audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
wati dongosolo layamba kale ndipo chimanga chifika m'misika ya deralo. A Chiponda adali mlendo wolemekezeka pa mwambowu
wati dongosolo layamba kale ndipo chimanga chifika m'misika ya deralo. A Chiponda adali mlendo wolemekezeka pa mwambowu
female
Gogo wa zaka 85, Alefa Pindani wa m'mudzi mwa Sale kudera la mfumu yaikulu Chiwalo ku Machinga
Gogo wa zaka eyite faifi, Alefa Pindani wa m'mudzi mwa Sale kudera la mfumu yaikulu Chiwalo ku Machinga
female
tsopano wapeza chakudya cha masiku akubwerawa kupyolera ku thandizo la chimanga lomwe boma, kudzera mu nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya Dodma
tsopano wapeza chakudya cha masiku akubwerawa kupyolera ku thandizo la chimanga lomwe boma, kudzera mu nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya Dodima
female
likupereka kwa mabanja okhudzidwa ndi Njala m’bomali. Polankhula atalandira thandizoli pomwe Dodma imagawa chimanga kwa anthu akudera la mfumu Chiwalo
likupereka kwa mabanja okhudzidwa ndi Njala m’bomali. Polankhula atalandira thandizoli pomwe Dodima imagawa chimanga kwa anthu akudera la mfumu Chiwalo
female
Gogo Pindani ati thandizoli labwera munthawi yake pomwe akuvutika ndi vuto la njala, ponena kuti amasowa ndalama zogulira chimanga chomwe chakwera mtengo kwambiri
Gogo Pindani ati thandizoli labwera munthawi yake pomwe akuvutika ndi vuto la njala, ponena kuti amasowa ndalama zogulira chimanga chomwe chakwera mtengo kwambiri
female
Ndipo DC waboma la Machinga a Rodrick Mateuma wati thandizoli likufikira mabanja 48,000 a m'bomali ndipo wapempha anthu omwe akupindula nawo mu ndondomekoyi kuti asagulitse chimangachi
Ndipo Disi waboma la Machinga a Rodiliki Mateuma wati thandizoli likufikira mabanja fote eyiti sauzande a m'bomali ndipo wapempha anthu omwe akupindula nawo mu ndondomekoyi kuti asagulitse chimangachi
female
Boma la Machinga ndi limodzi mwa maboma omwe adakhudzidwa ndi njala mu ulimi wa m'chaka cha 2022-2023 kutsatira Namondwe wa Freddy yemwe adakokolola mbewu zochuluka m'bomali
Boma la Machinga ndi limodzi mwa maboma omwe adakhudzidwa ndi njala mu ulimi wa m'chaka cha twente twente thu – twente twente fili kutsatira Namondwe wa Fulede yemwe adakokolola mbewu zochuluka m'bomali
female
Apolisi ku Lilongwe amanga abambo awiri omwe akuwaganizira kuti akhala akunamizira kuchita malonda a Taxi ndi cholinga chofuna kubera anthu
Apolisi ku Lilongwe amanga abambo awiri omwe akuwaganizira kuti akhala akunamizira kuchita malonda a Takisi ndi cholinga chofuna kubera anthu
female
Mneneri wa Polisi ku Lilongwe a Hastings Chigalu wati awiriwa ndi a Alick Kazembe a zaka 42, ochoka m'boma la Mangochi, komanso a Moses Mponda a zaka 35 ochoka ku Lilongwe
Mneneri wa Polisi ku Lilongwe a Hasiting’izi Chigalu wati awiriwa ndi a Aliki Kazembe a zaka fote thu, ochoka m'boma la Mangochi, komanso a Mozesi Mponda a zaka fete faifi ochoka ku Lilongwe
female
Awiriwa akuuti adanyamula bambo wina pa MRA ku Lilongwe kupita kwa Kabudula koma atafika pa Balon adamutsitsa bamboyo ndikumubera katundu wosiyanasiyana yense wokwana K700,000
Awiriwa akuuti adanyamula bambo wina pa Emu Ara Ee ku Lilongwe kupita kwa Kabudula koma atafika pa Baloni adamutsitsa bamboyo ndikumubera katundu wosiyanasiyana yense wokwana Seveni handede sauzande kwacha
female
A Chigalu ati awiriwa apezekanso ndi ma satifiketi monga a MSCE, Diploma ndi ma satifiketi ena a chipatala komanso zovala ndi katundu wina
A Chigalu ati awiriwa apezekanso ndi ma satifiketi monga a Emu esi si iii, Dipuloma ndi ma satifiketi ena a chipatala komanso zovala ndi katundu wina
Female
Anthuwa malinga ndi a Chigalu amagwiritsa ntchito galimoto ya mtundu wa Swift LA 8788 ndipo amachita izi ndi azawo ena awiri omwe apolisi akuwasakabe
Anthuwa malinga ndi a Chigalu amagwiritsa ntchito galimoto ya mtundu wa Swifuti Elo e eiti seveni eiti eiti ndipo amachita izi ndi azawo ena awiri omwe apolisi akuwasakabe
Female
Gulu la alimi a ng'ombe za mkaka okwana 500 la Mangunda m'boma la Thyolo lati lili ndi chiyembekezo kuti ndalama zokwana 5 million kwacha
Gulu la alimi a ng'ombe za mkaka okwana faifi handiledi la Mangunda m'boma la Thyolo lati lili ndi chiyembekezo kuti ndalama zokwana faifi miliyoni kwacha
Female
zomwe akhala akutaya pa mwezi kutsatira kuonongeka kwa mkaka kaamba ka kuzimazima kwa magetsi tsopano ikhala mbiri chabe
zomwe akhala akutaya pa mwezi kutsatira kuonongeka kwa mkaka kaamba ka kuzimazima kwa magetsi tsopano ikhala mbiri chabe
Female
Eliyasi Pirungu, yemwe ndi msungichuma wagululi wayankhula izi pomwe Transforming Agriculture Through Diversification and Entrepreneurship yapereka ndalama zokwana K107 million kwa alimiwa
Eliyasi Pirungu, yemwe ndi msungichuma wagululi wayankhula izi pomwe thilansifoming’I agilikacha fulu daivesifikeshoni and intapulinyuwashipi yapereka ndalama zokwana wani handedi andi seveni miliyoni kwacha kwa alimiwa
Female
zomwe akuti agwiritsa ntchito yogulira zipangizo zamagetsi zamakono za mphamvu ya dzuwa, komanso tank yosungira madzi
zomwe akuti agwiritsa ntchito yogulira zipangizo zamagetsi zamakono za mphamvu ya dzuwa, komanso thanki yosungira madzi
Female
Iwo ati akuyembekezera kugawa ndalama zokwana 20 million za dziko la America kupyolera mu ndondomekoyi
Iwo ati akuyembekezera kugawa ndalama zokwana Twente miliyoni za dziko la Amelika kupyolera mu ndondomekoyi
Female
President wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers a Thomson Mpinganjira wasankha board yatsopano Mu board yo muli iwo eni, komanso president wakale wa Bungwe la Sulom a Tiya Somba Banda, mwa anthu ena atsopano
Pulezidenti wa timu ya Maite Mukuru wandilazi a Thomusoni Mpinganjira wasankha bodi yatsopano Mu bodi yo muli iwo eni, komanso pulezidenti wakale wa Bungwe la Sulomu a Tiya Somba Banda, mwa anthu ena atsopano
Female
Ena mwa adindo atsopanowa ndi ma lawyer awiri a Chancy Gondwe ndi a David Kanyenda, kuphatikizapo a Madalitso Musa ndi Andre Kalinde
Ena mwa adindo atsopanowa ndi ma loya awiri a Tchanse Gondwe ndi a Devidi Kanyenda, kuphatikizapo a Madalitso Musa ndi Andile Kalinde
Female
Ndipo anthu ena akale mu board yi ndi a Limbani Magomelo ndi a Mervis Mangulenje
Ndipo anthu ena akale mu bodi yi ndi a Limbani Magomelo ndi a Mevisi Mangulenje
Female
Pamene kwangotsala tsiku limodzi kuti team ya mpira wa manja ya Civonets iyambe zokonzera zake mawa, Loweruka pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe, mphunzitsi wamkulu wa team yi a Whyte Mulilima wabangula
Pamene kwangotsala tsiku limodzi kuti timu ya mpira wa manja ya sivonetsi iyambe zokonzera zake mawa, Loweruka pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe, mphunzitsi wamkulu wa team yi a waiti Mulilima wabangula
Female
Mkuluyu wachenjeza team ya Blue Eagles sisters yomwe yakhala ikuwapanilira ma team anzake potenga ukatswiri wa m'chigawo cha pakati kuti nthawi yawo yatha tsopano
Mkuluyu wachenjeza team ya Blue Eagles sisters yomwe yakhala ikuwapanilira ma team anzake potenga ukatswiri wa m'chigawo cha pakati kuti nthawi yawo yatha tsopano
Female
Mulilima wati chaka chino, team yake ya Civonets itenga ukatswiri wa ligi. Mtsogoleri wakale wa ochemelera timu ya Mighty Mukuru Wanderers Yona 'Green' Malunga
Mulilima wati chaka chino, timu yake ya sivonetsi itenga ukatswiri wa ligi. Mtsogoleri wakale wa ochemelera timu ya maite Mukuru Wandilazi Yona 'Gilini' Malunga
Female
wati sizoni ya chaka chatha inali yowawa ku timuyi italephera potenga chikho
wati sizoni ya chaka chatha inali yowawa ku timuyi italephera potenga chikho
Female
Bwalo la milandu ku Mchinji lalamula abambo awiri kuti alipire chindapusa cha K50,000 aliyense chifukwa chong'amba ndalama ya K5000
Bwalo la milandu ku Mchinji lalamula abambo awiri kuti alipire chindapusa cha fifite sauzande kwacha aliyense chifukwa chong'amba ndalama ya faifi sauzande kwacha
Female
Mneneri wa polisi ya Mchinji a Limbani Mpinganjira wauza Times 360 Malawi kuti apolisi a kwa Kamwendo m'bomali adanjata anthuwa omwe ndi a Tsanzo Likisho
Mneneri wa polisi ya Mchinji a Limbani Mpinganjira wauza Taimusi fili sikisite Malawi kuti apolisi a kwa Kamwendo m'bomali adanjata anthuwa omwe ndi a Tsanzo Likisho
Female
komanso a Kelvin Elard, onse a zaka 23 zakubadwa, pa 27 December atang'amba ndalamayi ndi cholinga chakuti agawane
komanso a kelevini eladi, onse a zaka twente filii zakubadwa, pa twente seveni disemba atang'amba ndalamayi ndi cholinga chakuti agawane
Female
Malingana ndi a Mpinganjira, wapolisi wozenga milandu a Peter Fuluwenza adauza bwalo la milandu kuti awiriwa atalephera kugawana bwinobwino ndalamayi adagwirizana kuti angoing'amba pakati
Malingana ndi a Mpinganjira, wapolisi wozenga milandu a Pita Fuluwenza adauza bwalo la milandu kuti awiriwa atalephera kugawana bwinobwino ndalamayi adagwirizana kuti angoing'amba pakati
Female
kuti aliyense atenge gawo lake Awiriwa adakana mulanduwu zomwe zidachititsa mbali yaboma kuti ibweretse mboni zitatu
kuti aliyense atenge gawo lake Awiriwa adakana mulanduwu zomwe zidachititsa mbali yaboma kuti ibweretse mboni zitatu
Female
A Fuluwenza adapempha bwalo kuti lipereke chilango chokhwima Kwa awiriwa kuti likhale phunziro kwa anthu ena omwe amaganiza mwa chibwana chotere
A Fuluwenza adapempha bwalo kuti lipereke chilango chokhwima Kwa awiriwa kuti likhale phunziro kwa anthu ena omwe amaganiza mwa chibwana chotere
Female
Ndipo m'chigamulo chake, woweluza milandu a Yohane Nkhata anagwirizana ndi a Fuluwenza ndipo alamula awiriwa kuti alipire K50,000 aliyense, ndipo kuti akalephera akaseweze jele kwa chaka chimodzi
Ndipo m'chigamulo chake, woweluza milandu a Yohane Nkhata anagwirizana ndi a Fuluwenza ndipo alamula awiriwa kuti alipire fifite sauzande kwacha aliyense, ndipo kuti akalephera akaseweze jele kwa chaka chimodzi
Female
Oyendetsa maminibus m'chigawo cha kummwera adandaula chifukwa cha kusowa kwa zitupa za oyendetsa galimoto
Oyendetsa maminibasi m'chigawo cha kummwera adandaula chifukwa cha kusowa kwa zitupa za oyendetsa galimoto
Female
Oimirira oyendetsa maminibus m'chigawochi a Evance Galasi ayankhula izi ku nyumba yachifumu ya Sanjika mu mzinda wa Blantyre pa kukumana kwawo ndi mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera
Oimirira oyendetsa maminibus m'chigawochi a Evansi Galasi ayankhula izi ku nyumba yachifumu ya Sanjika mu mzinda wa Bulantaya pa kukumana kwawo ndi mtsogoleri wa dziko lino a Lazalasi Chakwera
Female
A Galasi ati pakadali pano nthambi yoona za pa msewu ya Road Traffic ikumangopereka mapepala mmalo mwa ziphaso zenizeni
A Galasi ati pakadali pano nthambi yoona za pa msewu ya Rodi thilafiki ikumangopereka mapepala mmalo mwa ziphaso zenizeni
Female
Iwo ati akadakonda nthambiyi itayambiranso kupereka zitupa zenizeni chifukwa zitupa za mapepala sizimachedwa kung’ambika
Iwo ati akadakonda nthambiyi itayambiranso kupereka zitupa zenizeni chifukwa zitupa za mapepala sizimachedwa kung’ambika
Female
Apolisi atsimikiza kuti carpet komanso tenti zimene zidasowa dzulo m'boma la Mwanza zapezeka
Apolisi atsimikiza kuti kapeti komanso tenti zimene zidasowa dzulo m'boma la Mwanza zapezeka
Female
Woyankhulira apolisi a Peter Kalaya watsimikiza kuti amanga anthu awiri powaganizira kuti ndi amene anaba zinthuzi
Woyankhulira apolisi a Pita Kalaya watsimikiza kuti amanga anthu awiri powaganizira kuti ndi amene anaba zinthuzi
Female
A Kalaya ati anthuwa ndi a Lino Richard komanso a Jonas Harold, onse a zaka makumi awiri
A Kalaya ati anthuwa ndi a Lino Litchadi komanso a Jonasi Halodi, onse a zaka makumi awiri
Female
Kummawaku zidamveka kuti carpet imene amayendapo mtsogoleri wa dziko komanso tenti zabedwa dzulo usiku koma a Kalaya adati zimene zinabedwazo ndi zinthu zina za mu unduna wa za mtengatenga
Kummawaku zidamveka kuti capeti imene amayendapo mtsogoleri wa dziko komanso tenti zabedwa dzulo usiku koma a Kalaya adati zimene zinabedwazo ndi zinthu zina za mu unduna wa za mtengatenga
Female
Mkulu woyang'anira ntchito za madzi m'boma la Mchinji a Ganizani Chilindanji walimbikitsa anthu okhala m'bomali kuti azimanga zimbudzi za makono zomwe amati Mwamuna apumule ati kamba ka lowe m'bomali

A Chilindanji amayankhula izi pa sukulu ya pulaimale ya Chitunda pomwe nthambi ya bungwe lowona ntchito za chitukuko ndi ukhondo la Assemblies of God Care ikuchita mderali
A Chilindanji amayankhula izi pa sukulu ya pulaimale ya Chitunda pomwe nthambi ya bungwe lowona ntchito za chitukuko ndi ukhondo la ambulesi ofu godi keya ikuchita mderali
Female
Iwo akuchita izi ndi thandizo la chuma lochokera ku Royal Norwegian Embassy kudzera mu bungwe la Norwegian Church Aid ndi Danish Church Aid
Iwo akuchita izi ndi thandizo la chuma lochokera ku Royo nowejiyani embase kudzera mu bungwe la Nowejiyani tchetchi edi ndi Danishi tchetchi edi
Female
Mmodzi wa anthu omwe apindula ndi zimbuzi zamakonozi a Paulo Mpenuka a zaka 37, ati amangitsa okha ndi ndalama zokwana k60,000
Mmodzi wa anthu omwe apindula ndi zimbuzi zamakonozi a Paulo Mpenuka a zaka fete seveni, ati amangitsa okha ndi ndalama zokwana sikisite sauzande kwacha
Female
ati amangitsa okha ndi ndalama zokwana k60,000 ati zimbuzi zake sizinunkha
ati amangitsa okha ndi ndalama zokwana sikisite sauzande kwacha ati zimbuzi zake sizinunkha
Female
komaso kuti pulojekiti-yi ithandiza ku nkhani za ukhondo pomwe anthu ayamba kusintha maganizo opotoka odzithandizira ku ntchire
komaso kuti pulojekitiyi ithandiza ku nkhani za ukhondo pomwe anthu ayamba kusintha maganizo opotoka odzithandizira ku ntchire
Female
Bwalo la milandu ku Zomba lagamula yemwe adali mfumu Mkwanda ya kwa Chikowi m'bomali kuti akakhale kundende kwa zaka 18 kaamba kogwilira mtsikana wa zaka 13
Bwalo la milandu ku Zomba lagamula yemwe adali mfumu Mkwanda ya kwa Chikowi m'bomali kuti akakhale kundende kwa zaka eitini kaamba kogwilira mtsikana wa zaka fetini
Female
A Lobin Katunga a zaka 52, atabwera ku bwalo la milandu, adakana mlanduwu
A Lobini Katunga a zaka fifite thu, atabwera ku bwalo la milandu, adakana mlanduwu
Female
Koma malinga ndi mboni zisanu zomwe a mbali yaboma motsogozedwa ndi a Lloyd Kachotsa aku polisi ya m'chigawo cha kumvuma adabweretsa, mkuluyu amupeza wolakwa
Koma malinga ndi mboni zisanu zomwe a mbali yaboma motsogozedwa ndi a Loyidi Kachotsa aku polisi ya m'chigawo cha kumvuma adabweretsa, mkuluyu amupeza wolakwa
Female
Zina mwa mbonizi, zidauza bwalo la milandu kuti mtsikanayu, yemwe sitimutchula dzina, ankayenda motsimphina
Zina mwa mbonizi, zidauza bwalo la milandu kuti mtsikanayu, yemwe sitimutchula dzina, ankayenda motsimphina
Female
Aphunzitsi ake atadabwa za izi adatengana ndi makolo ake a mtsikanayu ndipo adamutengera ku chipatala chachikulu ku Zomba, komwe adakatsimikiza kuti adali atamugwilira
Aphunzitsi ake atadabwa za izi adatengana ndi makolo ake a mtsikanayu ndipo adamutengera ku chipatala chachikulu ku Zomba, komwe adakatsimikiza kuti adali atamugwilira
Female
M'malo mwake, oweruza Milandu m'bwalo la Principal Resident Magistrate ku Zomba, a Martin Chipofya, agamula kuti mkuluyu akakhale ku ndende kwa zaka 18
M'malo mwake, oweruza Milandu m'bwalo la pulinsipo lezidenti majesitileti ku Zomba, a Matini Chipofya, agamula kuti mkuluyu akakhale ku ndende kwa zaka 18
Female
Ofesi yoona za chisamaliro cha anthu ku Neno yachenjeza kut idzagwiritsa ntchito lamulo popereka chilango kwa makolo omwe amatailira posapereka chisamaliro chokwanira kwa ana awo
Ofesi yoona za chisamaliro cha anthu ku Neno yachenjeza kut idzagwiritsa ntchito lamulo popereka chilango kwa makolo omwe amatailira posapereka chisamaliro chokwanira kwa ana awo
Female
Mkulu ku ofesi yoona za chisamarilo cha anthu m'bomali a Paul Sosono amayankhula izi pomwe gulu la anthu akufuna kwabwino m’bomali
Mkulu ku ofesi yoona za chisamarilo cha anthu m'bomali a Po Sosono amayankhula izi pomwe gulu la anthu akufuna kwabwino m’bomali
Female
limapereka thandizo la zinthu zosiyanasiyana kwa mwana wina wazaka 5 yemwe wanyentchera kaamba kosowa chisamarilo chokwanira
limapereka thandizo la zinthu zosiyanasiyana kwa mwana wina wazaka faifi yemwe wanyentchera kaamba kosowa chisamarilo chokwanira
Female
Mayi a mwanayu adamusiya ndi agogo ake ndi kupita ku Mozambique, komwe akuti amakachita bizinezi yogulitsa thupi, kaamba ka umphawi, ponena kuti bambo a mwanayu adamukana
Mayi a mwanayu adamusiya ndi agogo ake ndi kupita ku Mozambiki, komwe akuti amakachita bizinezi yogulitsa thupi, kaamba ka umphawi, ponena kuti bambo a mwanayu adamukana
Female
Koma mayiyu walonjeza kuti tsopano apereka chisamarilo kwa mwanayu kuti akule ndi thanzi
Koma mayiyu walonjeza kuti tsopano apereka chisamarilo kwa mwanayu kuti akule ndi thanzi
Female
Pamene boma lili palikulimbana ndi kufala kwa matenda a kolera m'dziko muno, Times 360 Malawi yapeza kuti Chipatala chaching'ono cha Lipili m'boma la Dowa chilibe chimbudzi ngakhale chimodzi
Pamene boma lili palikulimbana ndi kufala kwa matenda a kolera m'dziko muno, Taimusi fili sikisite Malawi yapeza kuti Chipatala chaching'ono cha Lipili m'boma la Dowa chilibe chimbudzi ngakhale chimodzi
Female
M'modzi wa anthu ogwira ntchito yongodzipereka pa chipatalachi, a Patrick Kawale, wati ndi zodandaulitsa kuona kuti anthu pa chipatalachi akumasowa kopita m'matupi mwawo mukatentha
M'modzi wa anthu ogwira ntchito yongodzipereka pa chipatalachi, a Patiliki Kawale, wati ndi zodandaulitsa kuona kuti anthu pa chipatalachi akumasowa kopita m'matupi mwawo mukatentha
Female
Mayi Florida Jimu wochokera m'mudzimwa mfumu Kachiwale m'dera la mfumu yayikulu Kayembe m'bomali wati miyoyo yawo ili pachippsyezo chotenga matenda a Kolera
Mayi Fulolida Jimu wochokera m'mudzimwa mfumu Kachiwale m'dera la mfumu yayikulu Kayembe m'bomali wati miyoyo yawo ili pachippsyezo chotenga matenda a Kolera
Female
Mneneri wa chipatala chachikulu cha Dowa, a Davie Nuka wati ofesi yawo ikudziwa za vutoli
Mneneri wa chipatala chachikulu cha Dowa, a Devi Nuka wati ofesi yawo ikudziwa za vutoli
Female
ndipo pakadali pano akuchita zothekera kuti pofika loweruka likubwerali, akhala atakumba ndi kumanga zimbudzi pamalopa
ndipo pakadali pano akuchita zothekera kuti pofika loweruka likubwerali, akhala atakumba ndi kumanga zimbudzi pamalopa
Female
Oweruza milandu a Madalitso Khoswe Chimwaza ati basi mlanduwu supitilira kumvedwa lero chifukwa sangapitilire kuwakakamiza a Buluma kuti apelekere umboni
Oweruza milandu a Madalitso Khoswe Chimwaza ati basi mlanduwu supitilira kumvedwa lero chifukwa sangapitilire kuwakakamiza a Buluma kuti apelekere umboni
Female
A Chimwaza ati zachitika lero n'zokhumudwitsa chifukwa a Buluma lero adafika m'bwaloli. A mbali yaboma auzidwa kuti abweretse lipoti lakuchipatala losonyeza kuti a Buluma akudwala
A Chimwaza ati zachitika lero n'zokhumudwitsa chifukwa a Buluma lero adafika m'bwaloli. A mbali yaboma auzidwa kuti abweretse lipoti lakuchipatala losonyeza kuti a Buluma akudwala
Female
Oweruza ati mbali zonse pa nkhaniyi zigwirizane kuti mlanduwu ubwerenso liti, a Buluma akapeze bwino
Oweruza ati mbali zonse pa nkhaniyi zigwirizane kuti mlanduwu ubwerenso liti, a Buluma akapeze bwino
Female
Oweruza milandu ku bwalo la Magistrate a Madalitso Khoswe Chimwaza akana pempho la mbali yaboma omwe amapempha bwaloli kuti liyimitse kaye mlandu wokhudza nduna yakale yoona za mphamvu a Newton Kambala ndi ena
Oweruza milandu ku bwalo la Majesitileti a Madalitso Khoswe Chimwaza akana pempho la mbali yaboma omwe amapempha bwaloli kuti liyimitse kaye mlandu wokhudza nduna yakale yoona za mphamvu a Nyutoni Kambala ndi ena
Female
Mkulu wa ACB a Martha Chizuma adapempha kuti mlanduwu uyimitsidwe kaye ponena kuti mboni ya boma a Helen Buluma sali okonzeka kupitilira kupelekera umboni m'bwaloli
Mkulu wa ESIBI a Mafa Chizuma adapempha kuti mlanduwu uyimitsidwe kaye ponena kuti mboni ya boma a Heleni Buluma sali okonzeka kupitilira kupelekera umboni m'bwaloli
Female
Koma oweruza a Chimwaza ati a mbali ya boma sadapereke zifukwa zokwanira pa pempho lawo ndipo ati ngati a Buluma atopa kutsatira kuima kwambiri m'bwaloli, apitilire kupereka umboni wawo atakhala pansi

Koma a Martha Chizuma apemphabe bwaloli kuti a Buluma sakwanitsa kupereka umboni m'bwaloli lero ponena kuti sali bwino
Koma a Mafa Chizuma apemphabe bwaloli kuti a Buluma sakwanitsa kupereka umboni m'bwaloli lero ponena kuti sali bwino
Female
Iwo ati a Buluma pa nthawi yomwe anali panja pa bwaloli adali akunjenjemera kusonyeza kuti sali bwino, a Chizuma adaonjezera kuti iwo aona izi ngakhale sali wachipatala
Iwo ati a Buluma pa nthawi yomwe anali panja pa bwaloli adali akunjenjemera kusonyeza kuti sali bwino, a Chizuma adaonjezera kuti iwo aona izi ngakhale sali wachipatala
Female
Koma woyimira mbali ya oyankhapo mlandu a Khumbo Soko ati a Buluma akunamizira kudwala chifukwa akuopa mafunso
Koma woyimira mbali ya oyankhapo mlandu a Khumbo Soko ati a Buluma akunamizira kudwala chifukwa akuopa mafunso
Female
Woyimira mbali ya oyankhapo mlandu ena a Wapona Kita adabwa kuti a Buluma ayamba kudwala nthawi zanji pomwe mphindi zochepa zapitazi adali akuyendayenda pa bwaloli
Woyimira mbali ya oyankhapo mlandu ena a Wapona Kita adabwa kuti a Buluma ayamba kudwala nthawi zanji pomwe mphindi zochepa zapitazi adali akuyendayenda pa bwaloli
Female
ndipo apempha bwalo kuti lingowamasula a Kambala, a Chihana ndi a Chaima. A Kambala, mtsogoleri wa chipani cha Aford a Enock Chihana ndi yemwe anali othandizira ntchito mtsogoleri wa dziko lino a Chris Chaima
ndipo apempha bwalo kuti lingowamasula a Kambala, a Chihana ndi a Chaima. A Kambala, mtsogoleri wa chipani cha Afodi a Inoki Chihana ndi yemwe anali othandizira ntchito mtsogoleri wa dziko lino a Khilisi Chaima
Female
anali othandizira ntchito mtsogoleri wa dziko lino a Chris Chaima ali m'bwaloli pa mlandu wawo wolowelera ntchito za mafuta a galimoto
anali othandizira ntchito mtsogoleri wa dziko lino a khilisi Chaima ali m'bwaloli pa mlandu wawo wolowelera ntchito za mafuta a galimoto
Female
ndipo a Buluma, omwe anali wachiwiri kwa mkulu wa bungwe la Nocma amayenera kupitilira kupeleka umboni pa nkhaniyi
ndipo a Buluma, omwe anali wachiwiri kwa mkulu wa bungwe la Nokoma amayenera kupitilira kupeleka umboni pa nkhaniyi
Female
Mtsogoleri wa anyamata osewera mu timu ya FCB Nyasa Big Bullets Precious Sambani wati ngakhale kuvulala kwake kwa pafupi pafupi kukudabwitsa
Mtsogoleri wa anyamata osewera mu timu ya Efu sibi Nyasa Bigi Buletsi Puleshasi Sambani wati ngakhale kuvulala kwake kwa pafupi pafupi kukudabwitsa
Female
iye akukhulupilira kuti adzabweleranso kukatenga malo ake mutimu yaikulu ya masewero a mpira wamiyendo yadziko lino
iye akukhulupilira kuti adzabweleranso kukatenga malo ake mutimu yaikulu ya masewero a mpira wamiyendo yadziko lino
Female
Sambani watha pafupifupi chaka ndi theka osasewelera timu ya Flames kamba kovulala, zimene zidachititsa kuti osewera mzake
Sambani watha pafupifupi chaka ndi theka osasewelera timu ya Fulemusi kamba kovulala, zimene zidachititsa kuti osewera mzake
Female
wa Bullets Alick Lungu atenge malo ake a otchinga kumbuyo kumanzere, koma naye Lungu sadachedwenso kuvulala ndipo pakadali pano, malowa akusewera ndi Tatenda M'balaka wa Silver Strikers
wa Buletsi Aliki Lungu atenge malo ake a otchinga kumbuyo kumanzere, koma naye Lungu sadachedwenso kuvulala ndipo pakadali pano, malowa akusewera ndi Tatenda M'balaka wa Siliva Sitilaikazi
Female
Iye wati akudabwa ndi kuvulala kumene amakumana nako, makamaka akamakonzekera masewero a ku kalabu kwake, ngakhale ku national team
Iye wati akudabwa ndi kuvulala kumene amakumana nako, makamaka akamakonzekera masewero a ku kalabu kwake, ngakhale ku neshono timu
Female
A Khumbo Soko ati a Buluma ndi mbali ya boma ali ndi mantha ndipo n'chifukwa chake akufuna mlanduwu usapitilire kumvedwa lero
A Khumbo Soko ati a Buluma ndi mbali ya boma ali ndi mantha ndipo n'chifukwa chake akufuna mlanduwu usapitilire kumvedwa lero
Female
Iwo ati, mboni imafunsidwa mafunso ovuta ndi maloya mpaka mboniyo kutenthedwa kumene, koma izi sizitanthauza kuti mlanduwo uyime kaye mpaka mboni itakazizidwako
Iwo ati, mboni imafunsidwa mafunso ovuta ndi maloya mpaka mboniyo kutenthedwa kumene, koma izi sizitanthauza kuti mlanduwo uyime kaye mpaka mboni itakazizidwako
Female
A Soko ati aona kale kuti a Buluma atenthedwa ndipo akungofuna kukapitidwa mphepo koma ati ichi sichifukwa chokwanira kuti mpaka kufunsidwa kwawo kwa mafunso kuyime
A Soko ati aona kale kuti a Buluma atenthedwa ndipo akungofuna kukapitidwa mphepo koma ati ichi sichifukwa chokwanira kuti mpaka kufunsidwa kwawo kwa mafunso kuyime
Female
Iwo apereka chitsanzo cha milandu ina pomwe mboni inafika potulutsa msozi. zimene m'Chichewa zikutanthauza kuti, mboni ina inalira pa bwalo la milandu
Iwo apereka chitsanzo cha milandu ina pomwe mboni inafika potulutsa msozi. zimene m'Chichewa zikutanthauza kuti, mboni ina inalira pa bwalo la milandu
Female
koma bwalo silinayimitse kuti basi mboniyo isafunsidwenso mafunso
koma bwalo silinayimitse kuti basi mboniyo isafunsidwenso mafunso
Female
A Soko ati bwalo lisalore kuti kumvedwa kwa mlanduwu kuyimitsidwe chifukwa ACB siikupereka chifukwa chomveka
A Soko ati bwalo lisalore kuti kumvedwa kwa mlanduwu kuyimitsidwe chifukwa Esi bii siikupereka chifukwa chomveka
Female
Koma a Martha Chizuma ati bwalo limve pempho lawo, chifukwa oyankhapo mlandu nawo m'mbuyomu apemphapo kuti mlandu uyimitsidwe ndipo bwalo linkawamvetsera
Koma a Mafa Chizuma ati bwalo limve pempho lawo, chifukwa oyankhapo mlandu nawo m'mbuyomu apemphapo kuti mlandu uyimitsidwe ndipo bwalo linkawamvetsera
Female
Mkulu wa bungwe lothana ndi katangale la ACB a Martha Chizuma wapempha bwalo kuti liyambe laimitsa kaye mlanduwu
Mkulu wa bungwe lothana ndi katangale la Esi bii a Mafa Chizuma wapempha bwalo kuti liyambe laimitsa kaye mlanduwu
Female
ponena kuti mboni ya mbali ya boma a Helen Buluma sali okonzeka kupitilira kupelekera umboni lero
ponena kuti mboni ya mbali ya boma a Heleni Buluma sali okonzeka kupitilira kupelekera umboni lero
Female
Iwo ati ngakhale a Buluma abwera mu bwaloli lero, sali moyenelera kupitilira kupelekera umboni kotero ambali ya boma akufuna mlanduwu uyimitsidwe kaye
Iwo ati ngakhale a Buluma abwera mu bwaloli lero, sali moyenelera kupitilira kupelekera umboni kotero ambali ya boma akufuna mlanduwu uyimitsidwe kaye
Female
A Chizuma ati, ngakhale ozengedwa mlandu ali ndi ufulu woti mlandu wawo umvedwe moyenelera, palinso kufunikira kuti a mbali ya boma adzipatsidwa mwayi ndi mpata wozenga mlandu munjira yomwe sakupsinjika

Koma woyimira mbali ya oyankhapo mlandu a Wapona Kita adabwa kuti n'chifukwa chani a mbali ya boma akufuna mlanduwu uyimitsidwe pomwe a Buluma ali kale m'bwaloli
Koma woyimira mbali ya oyankhapo mlandu a Wapona Kita adabwa kuti n'chifukwa chani a mbali ya boma akufuna mlanduwu uyimitsidwe pomwe a Buluma ali kale m'bwaloli
Female
Adafunsa motero a Kita uku atatembenuka kuwayang'ana a Buluma omwe akhala kumbuyo ndi ena odzamvera mlanduwu
Adafunsa motero a Kita uku atatembenuka kuwayang'ana a Buluma omwe akhala kumbuyo ndi ena odzamvera mlanduwu
Female
Woyimira mbali ya oyankhapo mlandu a Khumbo Soko atinso mbali ya boma inene zifukwa zomwe sali okonzeka kupitilira ndi mlanduwu lero
Woyimira mbali ya oyankhapo mlandu a Khumbo Soko atinso mbali ya boma inene zifukwa zomwe sali okonzeka kupitilira ndi mlanduwu lero
Female
Boma lakhazikitsa malamulo atsopano a malipiro a ntchito m'dziko muno, omwe nduna yoona za ntchito a Agnes Nyalonje alamula kuti ayambe kugwiritsidwa ntchito kuyambira pa 1 February
Boma lakhazikitsa malamulo atsopano a malipiro a ntchito m'dziko muno, omwe nduna yoona za ntchito a Aginesi Nyalonje alamula kuti ayambe kugwiritsidwa ntchito kuyambira pa 1 febuluwale
Female
Malamulowa akukhudza ogwira ntchito m'ma kampani ang'onoang'ono komanso madalaiva a galimoto zoyenda m'dziko muno komanso zopita m'maiko a kunja
Malamulowa akukhudza ogwira ntchito m'ma kampani ang'onoang'ono komanso madalaiva a galimoto zoyenda m'dziko muno komanso zopita m'maiko a kunja
Female
Malinga ndi malamulo atsopanowa, malipiro asintha kuchoka pa K1,900 patsiku, yomwe inali K57,000 pa mwezi
Malinga ndi malamulo atsopanowa, malipiro asintha kuchoka pa wani sauzande naini hande kwacha patsiku, yomwe inali fifite seveni sauzande kwacha pa mwezi
Female
kufika pa K 3,000 patsiku yomwe ndi k 103, 000 kwacha pa mwezi kwa ogwira ntchito m'ma kampani okulilapo
kufika pa fili sauzande kwacha patsiku yomwe ndi wani handede andi filii sauzande kwacha pa mwezi kwa ogwira ntchito m'ma kampani okulilapo
Female
Kwa ogwira ntchito m'ma kampani ochepera, malipiro awo akwezedwa kufika pa K2,000 pa tsiku ndipo ogwira ntchito zapakhomo malipiro awo akwezedwa kufika pa K2,000 pa tsiku
Kwa ogwira ntchito m'ma kampani ochepera, malipiro awo akwezedwa kufika pa thu sauzande kwacha pa tsiku ndipo ogwira ntchito zapakhomo malipiro awo akwezedwa kufika pa pa thu sauzande kwacha pa tsiku
Female
yomwe ili K60,000 pa mwezi, malamulowa atinso ma dalaiva oyendetsa galimoto zing'onozing'ono akuyenera kulandira ndalama yosachepera K100,000
yomwe ili sikisite sauzande kwacha pa mwezi, malamulowa atinso ma dalaiva oyendetsa galimoto zing'onozing'ono akuyenera kulandira ndalama yosachepera wani handede sauzande kwacha
Female
akuyenera kulandira ndalama yosachepera K234,000
akuyenera kulandira ndalama yosachepera thu handede andi fete folo sauzande kwacha
Female