Datasets:
audio audioduration (s) 0.52 42.4 | text stringlengths 3 501 | duration float32 0.52 42.4 | score float64 -44.97 -0.06 |
|---|---|---|---|
ndipo yobu anayankha kuti, zoonadi, ndikudziwa kuti zimenezi ndi zoona. | 9.46 | -10.265566 | |
koma munthu angathe bwanji kukhala wolungama pamaso pa mulungu? | 5.38 | -6.654978 | |
ngakhale wina atafuna kutsutsana naye, iye sangamuyankhe munthuyo ngakhale mawu amodzi omwe. | 7.84 | -11.428797 | |
mulungu ndi wa nzeru zambiri ndipo mphamvu zake ndi zochuluka. | 5.08 | -3.513787 | |
ndani analimbana naye popanda kupwetekeka? | 4.34 | -2.180903 | |
iye amasuntha mapiri, mapiriwo osadziwa, ndipo amawagubuduza ali wokwiya. | 8.76 | -5.225481 | |
iye amagwedeza dziko lapansi kulisuntha pamalo pake ndipo amanjenjemeretsa mizati yake. | 7.96 | -9.40664 | |
iye amayankhula ndi dzuwa ndipo siliwala; iyeyo amaphimba kuwala kwa nyenyezi. | 9.24 | -8.134401 | |
ndi mulungu yekha amene anayala mayiko akumwamba ndipo amayenda pa mafunde a pa nyanja. | 8.82 | -2.439217 | |
iye ndiye mlengi wa nyenyezi zamlalangʼamba ndi akamwiniatsatana, nsangwe ndi kumpotosimpita. | 12.9 | -12.055559 | |
iye amachita zozizwitsa zimene sizimvetsetseka, zodabwitsa zimene sizingawerengeke. | 9.68 | -5.272598 | |
akapita pafupi ndi ine sindingathe kumuona; akadutsa, sindingathe kumuzindikira. | 6.8 | -14.689873 | |
ngati iye alanda zinthu, ndani angathe kumuletsa? | 4.6 | -3.346789 | |
ndani anganene kwa iye kuti, mukuchita chiyani? | 4.52 | -2.402993 | |
mulungu sabweza mkwiyo wake; ngakhale gulu lankhondo la rahabe linawerama pa mapazi ake. | 8.38 | -6.790832 | |
nanga ine ndingathe kukangana naye bwanji? | 3.54 | -6.217046 | |
ndingawapeze kuti mawu oti nʼkutsutsana naye? | 4.3 | -11.459249 | |
ngakhale nditakhala wosalakwa, sindingamuyankhe; ndikanangopempha chifundo kwa woweruza wanga. | 9.54 | -37.159729 | |
ngakhale ndikanamuyitana ndipo iye ndi kuvomera, sindikhulupirira kuti akanamva mawu angawo. | 8.8 | -34.67207 | |
iye akanandikantha ndi mphepo yamkuntho, ndipo akanandipweteka popanda chifukwa. | 8.72 | -27.760382 | |
mulungu sakanandilola kuti ndipumenso koma akanandichulukitsira zowawa. | 7.92 | -14.312737 | |
tikanena za mphamvu, iye ndi wamphamvudi! | 4.2 | -6.310073 | |
ndipo tikanena za chiweruzo cholungama, ndani angamuzenge mlandu? | 6.04 | -3.399483 | |
ngakhale ndikanakhala wosalakwa, zoyankhula zanga zikananditsutsa; ndikanakhala wopanda cholakwa, pakamwa panga pakanandipeza wolakwa. | 13.26 | -34.842247 | |
ngakhale ine ndili wosalakwa, sindidziyenereza ndekha; moyo wanga ndimawupeputsa. | 7.76 | -12.731842 | |
zonse nʼzofanana; nʼchifukwa chake ndikuti, iye amawononga anthu osalakwa ndi anthu oyipa omwe. | 9 | -43.252918 | |
pamene mkwapulo ubweretsa imfa yadzidzidzi, iye amaseka tsoka la munthu wosalakwayo. | 9.38 | -6.07876 | |
pamene dziko lagwa mʼmanja mwa anthu oyipa iye amawatseka maso anthu oweruza dzikolo. | 7.82 | -10.091639 | |
ngati si iyeyo, nanga ndani? | 3.24 | -2.390084 | |
masiku anga ndi othamanga kwambiri kupambana munthu waliwiro; masikuwo amapita ine osaonapo zabwino. | 9.88 | -14.1373 | |
amayenda ngati mabwato a njedza pa nyanja, ngati mphungu zothamangira nyama zoti zidye. | 8.06 | -19.31358 | |
nʼtanena kuti, ndidzayiwala madandawulo anga, ndidzasintha nkhope yanga ndipo ndidzasekerera, ndikuopabe mavuto anga onse, popeza ndikudziwa kuti simudzavomereza kuti ndine wosalakwa. | 16.219999 | -23.745808 | |
popeza ndapezeka kale wolakwa ndivutikirenji popanda phindu? | 6.4 | -20.734715 | |
ngakhale nditasamba mʼmadzi oyera kwambiri ndi kusamba mʼmanja mwanga ndi sopo, mutha kundiponyabe pa dzala, kotero kuti ngakhale zovala zanga zomwe zidzandinyansa. | 13.9 | -18.503939 | |
mulungu si munthu ngati ine kuti ndithe kumuyankha, sindingathe kutsutsana naye mʼbwalo la milandu. | 9.38 | -27.208384 | |
pakanapezeka munthu wina kuti akhale mʼkhalapakati wathu, kuti atibweretse ife tonse pamodzi, munthu wina woti achotse ndodo ya mulungu pa ine kuti kuopsa kwake kusandichititsenso mantha! | 18.34 | -20.179951 | |
pamenepo ine ndikanatha kuyankhula mosamuopa mulunguyo, koma monga zililimu, sindingathe. | 8.9 | -31.714552 | |
koma tsopano, yehova amene anakulenga, iwe yakobo, amene anakuwumba, iwe israeli akuti, usaope, pakuti ndakuwombola; ndinakuyitanitsa mokutchula dzina lako, ndiwe wanga. | 16.32 | -13.909834 | |
pamene ukuwoloka nyanja, ndidzakhala nawe; ndipo pamene ukuwoloka mitsinje, sidzakukokolola. | 7.58 | -6.157608 | |
pamene ukudutsa pa moto, sudzapsa; lawi la moto silidzakutentha. | 5.86 | -5.672008 | |
chifukwa ine yehova, mulungu wako, woyera wa israeli, ndine mpulumutsi wako. | 6.28 | -3.780488 | |
ndinapereka igupto pofuna kuti ndiwombole iwe, ndinapereka kusi ndi seba mʼmalo mwa iwe. | 7.68 | -6.856777 | |
popeza kuti ndiwe wamtengowapatali wolemekezeka ndi wapamtima panga, ndipo chifukwa ndimakukonda, ndidzapereka anthu mʼmalo mwa iwe, ndidzapereka mitundu ya anthu pofuna kuwombola moyo wako. | 15.92 | -20.042549 | |
usachite mantha, pakuti ine ndili nawe; ndidzabweretsa ana ako kuchokera kummawa, ndipo ndidzakusonkhanitsani kuchokera kumadzulo. | 9.62 | -24.249731 | |
ndidzawuza a kumpoto kuti, amasuleni, ndidzawuza akummwera kuti, musawagwire. | 7.02 | -3.722626 | |
bweretsani ana anga aamuna kuchokera ku mayiko akutali, ana anga a akazi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi; onsewo amadziwika ndi dzina langa; ndinawalenga chifukwa cha ulemerero wanga, ndinawawumba, inde ndinawapanga. | 17.82 | -15.021706 | |
tulutsa anthu amene ali nawo maso koma sakupenya, anthu amene ali nawo makutu koma sakumva. | 9.38 | -6.567092 | |
abweretu ndi mboni zawo kuti adzatsimikizire kuti ananena zoona, kuti anthu ena amve ndi kunena kuti, ndi zoona. | 9.32 | -6.079308 | |
yehova akunena kuti, inu aisraeli ndinu mboni zanga, ndi mtumiki wanga amene ndinakusankha, kuti mundidziwe ndi kundikhulupirira, ndipo mudzamvetsa kuti mulungu ndine ndekha. | 15.24 | -12.326422 | |
patsogolo panga sipanapangidwepo mulungu wina, ngakhale pambuyo panga sipadzakhalaponso wina. | 7.6 | -5.989388 | |
akutero yehova, ine, inetu ndine yehova, ndipo palibe mpulumutsi wina koma ine ndekha. | 8.3 | -6.39843 | |
ndine amene ndinaneneratu, amene ndinakupulumutsa; ndine, osati mulungu wina wachilendo pakati panu amene ndinalengezeratu. | 10.68 | -25.311016 | |
inu ndinu mboni zanga, kuti ine ndine mulungu, akutero yehova. | 6.02 | -1.781113 | |
ine ndine mulungu kuyambira nthawi yamakedzana, ndipo ndidzakhalabe mulungu ku nthawi zonse. | 6.42 | -2.984262 | |
palibe amene angathe kuthawa mʼmanja mwanga, ndipo chimene ndachita palibe angathe kuchisintha. | 7.64 | -5.764726 | |
yehova akuti, mpulumutsi wanu, woyerayo wa israeli akuti, chifukwa cha inu ndidzatuma gulu lankhondo kukalimbana ndi babuloni ndi kukupulumutsani. | 13.2 | -23.984167 | |
ndidzagwetsa zitseko zonse za mzindawo, ndipo kukondwa kwa anthu ake kudzasanduka kulira. | 7.98 | -4.85169 | |
ine ndine yehova, woyera wanu uja, mlengi wa israeli. | 5 | -4.582711 | |
ine ndine mfumu yanu. | 1.9 | -1.439109 | |
yehova anapanga njira pa nyanja, anapanga njira pakati pa madzi amphamvu. | 6.06 | -6.751146 | |
iye anasonkhanitsa magaleta, akavalo, gulu lankhondo ndi asilikali amphamvu, ndipo onse anagwa pamenepo, osadzukanso anazimitsidwa kutheratu ngati chingwe cha nyale. | 15.38 | -16.700905 | |
yehova ameneyu akuti, iwalani zinthu zakale; ndipo musaganizirenso zinthu zimene zinachitika kale. | 9.1 | -10.89904 | |
taonani, ine ndikuchita zinthu zatsopano! | 2.98 | -1.605354 | |
tsopano zayamba kale kuoneka; kodi simukuziona? | 4.72 | -4.501631 | |
ine ndikulambula msewu mʼchipululu ndi kupanga mitsinje mʼdziko lowuma. | 6.18 | -9.238358 | |
nyama zakuthengo, nkhandwe ndi akadzidzi zinandilemekeza. | 5.32 | -17.16884 | |
ndidzayendetsa mitsinje mʼdziko lowuma kuti ndiwapatse madzi anthu anga osankhidwa. | 7.34 | -7.804178 | |
anthu amene ndinadziwumbira ndekha kuti aziyimba nyimbo yotamanda ine. | 6.32 | -20.165384 | |
komatu simunapemphera kwa ine, inu a mʼbanja la yakobo, munatopa nane, inu aisraeli. | 8.98 | -4.666229 | |
simunabweretse kwa ine nkhosa za nsembe zopsereza, kapena kundilemekeza ndi nsembe zanu. | 7.5 | -20.211315 | |
ine sindinakulemetseni pomakupemphani zopereka za chakudya kapena kukutopetsani pomakupemphani nsembe zofukiza. | 10.84 | -16.132109 | |
simunandigulire bango lonunkhira kapena kundipatsa ine mafuta okwanira a nsembe zanu. | 7.02 | -6.159363 | |
koma inu mwandilemetsa ine ndi machimo anu ndipo mwanditopetsa ine ndi zolakwa zanu. | 7.4 | -8.668964 | |
ine, inetu, ndi amene ndimafafaniza zolakwa zanu, chifukwa cha ine mwini, ndipo sindidzakumbukiranso machimo anu. | 9.74 | -35.452236 | |
mundikumbutse zakale, ndipo titsutsane nkhaniyi pamodzi; fotokozani mlandu wanu kuti muonetse kuti ndinu osalakwa. | 9.6 | -12.706884 | |
kholo lanu loyamba linachimwa; ndipo atsogoleri anu achipembedzo anandiwukira. | 6.74 | -5.433934 | |
chifukwa chake ine ndidzanyazitsa akuluakulu a nyumba yanu ya mapemphero, ndipo ndidzapereka yakobo kuti awonongedwe ndi israeli kuti achitidwe chipongwe. | 12.36 | -14.941694 | |
ndimvereni yehova ndipo mundiyankhe, pakuti ndine wosauka ndi wosowa. | 5.2 | -16.135967 | |
yangʼanirani moyo wanga, pakuti ndine wodzipereka kwa inu. | 4 | -3.374545 | |
inu ndinu mulungu wanga; pulumutsani mtumiki wanu amene amadalira inu. | 5.88 | -6.524107 | |
inu ndinu mulungu wanga. | 1.54 | -5.839418 | |
mundichitire chifundo, inu ambuye, pakuti ndikuyitana inu tsiku lonse. | 5.06 | -7.658508 | |
bweretsani chimwemwe kwa mtumiki wanu, ambuye, pakuti ndimadalira inu. | 6.38 | -6.259902 | |
inu ambuye, ndinu wokhululuka ndi wabwino, wodzaza ndi chikondi kwa onse amene amayitana inu. | 7.54 | -8.489582 | |
yehova imvani pemphero langa; mvetserani kulira kwanga kofuna chifundo. | 5.86 | -14.820835 | |
pa tsiku la mavuto anga ndidzayitana inu, pakuti inu mudzandiyankha. | 5.78 | -10.310166 | |
pakati pa milungu palibe wina wofanana nanu ambuye; palibe ntchito zolingana ndi ntchito zanu. | 7.2 | -5.477332 | |
mitundu yonse ya anthu imene munayipanga idzabwera ndi kudzalambira pamaso panu ambuye; iwo adzabweretsa ulemerero pa dzina lanu. | 11.34 | -18.772198 | |
pakuti ndinu wamkulu ndipo mumachita zodabwitsa; inu nokha ndiye mulungu. | 6.14 | -8.116363 | |
ndiphunzitseni njira yanu yehova, ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu; patseni mtima wosagawikana kuti ndilemekeze dzina lanu. | 10.56 | -41.37598 | |
ndidzakutamandani ambuye mulungu wanga, ndi mtima wanga wonse; ndidzalemekeza dzina lanu kwamuyaya. | 7.62 | -12.131342 | |
pakuti chikondi chanu nʼchachikulu kwa ine; mwandipulumutsa ku malo ozama a manda. | 6.68 | -11.519662 | |
inu mulungu wanga, anthu odzikuza akundithira nkhondo; anthu ankhanza akufuna kundipha, amene salabadira za inu. | 11.6 | -13.544672 | |
koma ambuye ndinu mulungu wachifundo ndi wokoma mtima, wosakwiya msanga, wodzaza ndi chikondi ndi wokhulupirika. | 9.9 | -12.93224 | |
tembenukirani kwa ine ndipo ndichitireni chifundo; perekani mphamvu zanu kwa mtumiki wanu ndipo pulumutsani mwana wa mdzakazi wanu. | 12.62 | -16.678186 | |
mundionetse chizindikiro cha ubwino wanu kuti adani achione ndi kuchititsidwa manyazi, pakuti yehova mwandithandiza ndi kunditonthoza. | 11.86 | -17.971775 | |
mayiyo ananyamuka nachita zimene munthu wa mulungu ananena. | 5.68 | -5.135348 | |
iye pamodzi ndi banja lake anachoka nakakhala ku dziko la afilisti zaka zisanu ndi ziwiri. | 7.78 | -6.170766 | |
zitatha zaka zisanu ndi ziwirizo anabwera kuchokera ku dziko la afilisti ndipo anapita kwa mfumu kukafunsa za nyumba yake ndi munda wake. | 12.38 | -8.123016 | |
ndipo mfumu inkayankhula ndi gehazi, mtumiki wa munthu wa mulungu kuti, tandiwuza zinthu zikuluzikulu zimene elisa wachita. | 12.74 | -10.751536 |
BibleTTS Chichewa — Aligned Bible Speech
116.1 hours of studio-quality, single-speaker Chichewa Bible narration, segmented and force-aligned at verse level into 45,728 clips (24 kHz, mono, WAV).
Languages
nya— Chichewa or Chewa
Dataset Structure
Audio is stored in the audio column (HuggingFace Audio feature). Parquet shards live under data/read/, one file per split.
from datasets import load_dataset
ds = load_dataset("CLEAR-Global/BibleTTS-Chichewa", "read", split="train")
| field | description |
|---|---|
audio |
The clip. audio.path is the source file name, <BOOK>_<chapter>_<segment>.wav. |
text |
Verse transcript, lowercase. |
duration |
Clip duration in seconds. |
score |
Alignment confidence for the clip (see below). |
Statistics
| split | clips | hours | median / p95 duration (s) |
|---|---|---|---|
train |
40,150 | 100.81 | 8.2 / 17.8 |
dev |
249 | 0.76 | 10.5 / 21.0 |
test |
117 | 0.38 | 11.2 / 23.7 |
other |
5,212 | 14.15 | 7.2 / 26.6 |
| total | 45,728 | 116.10 | 8.1 / 18.8 |
The corpus has a single speaker (one recording voice) and no speaker or demographic metadata.
Splits and the Alignment Score
Each clip carries a score from the forced aligner: the alignment confidence for that clip, expressed as an average per-token log-probability. Values are negative; higher is better. It is length-normalised, so long and short clips are comparable, and it is not correlated with clip duration or transcript length.
Every clip is published in one of four splits. Nothing is discarded:
train/dev/test— the cleaned set (40,516 clips, 101.95 h). A clip is included only if it passes both filters:score > -45— alignment considered reliable; and- no numerals in the transcript — Chichewa verse text containing figures (
"…wa zaka '32'…") is kept out of the training splits because the numbers are spoken as words and do not match a plain-text transcript.
other— the 5,212 clips (14.15 h) excluded by those filters; not intended for TTS training as-is.
Dataset Creation
BibleTTS's Chichewa subset was published as unaligned chapter-level audio from Open.Bible released by Biblica. This release is the CLEAR Global verse-level segmentation of those recordings: each chapter was split into per-verse clips and force-aligned against the Chichewa Bible text, which yielded the per-clip transcripts, durations and alignment scores used here. Clips are 24 kHz mono PCM WAV.
Caveats
- Single speaker, Bible-domain vocabulary: not representative of everyday spoken Chichewa.
- Verse-level segmentation follows the Bible text; some clips are verse fragments, so transcripts are not always complete sentences.
- The
othersplit is deliberately unfiltered and therefore contains misaligned clips and transcripts with numerals.
Citation
@inproceedings{meyer22c_interspeech,
title = {{BibleTTS: a large, high-fidelity, multilingual, and uniquely African speech corpus}},
author = {Josh Meyer and David Adelani and Edresson Casanova and Alp Öktem and Daniel Whitenack and Julian Weber and Salomon {KABONGO KABENAMUALU} and Elizabeth Salesky and Iroro Orife and Colin Leong and Perez Ogayo and Chris {Chinenye Emezue} and Jonathan Mukiibi and Salomey Osei and Apelete AGBOLO and Victor Akinode and Bernard Opoku and Olanrewaju Samuel and Jesujoba Alabi and Shamsuddeen Hassan Muhammad},
year = {2022},
booktitle = {{Interspeech 2022}},
pages = {2383--2387},
doi = {10.21437/Interspeech.2022-10850},
issn = {2958-1796},
}
@inproceedings{derenzi-etal-2025-synthetic,
title = "Synthetic Voice Data for Automatic Speech Recognition in {A}frican Languages",
author = "DeRenzi, Brian and Dixon, Anna and Farhi, Mohamed Aymane and Resch, Christian",
booktitle = "Proceedings of the First Workshop on Advancing {NLP} for Low-Resource Languages",
month = sep,
year = "2025",
address = "Varna, Bulgaria",
publisher = "INCOMA Ltd., Shoumen, Bulgaria",
url = "https://aclanthology.org/2025.lowresnlp-1.16/",
pages = "152--186"
}
Contact
CLEAR Global — tech@clearglobal.org
Acknowledgments
Verse-level alignment and packaging by CLEAR Global, continuing the Masakhane BibleTTS collaboration. Original recordings from the Open.Bible project by Biblica.
License
CC BY-SA 4.0 (SPDX: cc-by-sa-4.0)
- Downloads last month
- 54