audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
aphungu asanayikambilane.Biluyi imaloleza boma kubwereka ndalama zokwana K 93 billion kuchokera ku bank ya Baroda ndipo cholinga chake akuti chinali kumangira nyumba za nthambi za chitetezo m’dziko muno | aphungu asanayikambilane.Biluyi imaloleza boma kubwereka ndalama zokwana nainte fili biliyonikwacha kuchokera ku banki ya Baroda ndipo cholinga chake akuti chinali kumangira nyumba za nthambi za chitetezo m’dziko muno | Female | |
Sabata yatha a polisi anamanga m’busa Martin Thom yemwe anali mlangizi wa padera wa President Lazarus Chakwera komanso komanso m’modzi mwa akuluakulu ku unduna wa za chuma a Nations Msowoya | Sabata yatha a polisi anamanga m’busa Matini Thomu yemwe anali mlangizi wa padera wa Pulezidenti Lazalasi Chakwera komanso komanso m’modzi mwa akuluakulu ku unduna wa za chuma a Neshonzi Msowoya | Female | |
powaganizira kuti akukhuzidwa ndi nkhaniyi. Apolisi ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre atsekera m’chitokosi mnyamata wina wa zaka 17 | powaganizira kuti akukhuzidwa ndi nkhaniyi. Apolisi ku Ndirande mu mzinda wa Bulantaya atsekera m’chitokosi mnyamata wina wa zaka seventini | Female | |
yemwe amachita business ya kabaza pomuganizira kuti wakhala akugwililira mpaka kupereka mimba kwa mwana za zaka 15 zakubadwa yemwe ndi ophunzira pa sukulu ina | yemwe amachita buzinezi ya kabaza pomuganizira kuti wakhala akugwililira mpaka kupereka mimba kwa mwana za zaka fifitini zakubadwa yemwe ndi ophunzira pa sukulu ina | Female | |
Malingana ndi mneneri wa polisi ya Ndirande, Kelvin Nyirenda, oganizilidwayu yemwe sitimutchula dzina pofuna kumuteteza ndi wa m'mudzi mwa Manama mfumu yaikulu Kapeni ku Blantyre komweko | Malingana ndi mneneri wa polisi ya Ndirande, Keovini Nyirenda, oganizilidwayu yemwe sitimutchula dzina pofuna kumuteteza ndi wa m'mudzi mwa Manama mfumu yaikulu Kapeni ku Bulantaya komweko | Female | |
Nyirenda wati apolisi auzidwa ndi mai ake a mtsikanayu kuti mwanayu sanaoneke pa khomo la kwawo kuchokera pa 31 July ndipo anabwelera pa khomo-li pa 3 August | Nyirenda wati apolisi auzidwa ndi mai ake a mtsikanayu kuti mwanayu sanaoneke pa khomo la kwawo kuchokera pa fete wani julayi ndipo anabwelera pa khomoli pa fili gasiti | Female | |
ndipo atamufunsa, anaulula kuti anali ku dera la Baghdad ku Ndirandeko komwe oganiziridwayu amakhala. Maiyu wauzanso apolisi kuti atapitiliza kumufunsa mafunso | ndipo atamufunsa, anaulula kuti anali ku dera la Bakidadi ku Ndirandeko komwe oganiziridwayu amakhala. Maiyu wauzanso apolisi kuti atapitiliza kumufunsa mafunso | Female | |
mwanayu anati ndi oyemebekezera poonjezera kuti wakhala akugonana mosaziteteza ndi mkuluyu kuyambira mwezi wa January chaka chino | mwanayu anati ndi oyemebekezera poonjezera kuti wakhala akugonana mosaziteteza ndi mkuluyu kuyambira mwezi wa Januwale chaka chino | Female | |
Apa, apolisi anamanga mkuluyu ndipo malingana ndi Nyirenda, aonekera ku bwalo la milandu posachedwapa kafukufuku wa apolisi pa nkhaniyi akafika ku mapeto | Apa, apolisi anamanga mkuluyu ndipo malingana ndi Nyirenda, aonekera ku bwalo la milandu posachedwapa kafukufuku wa apolisi pa nkhaniyi akafika ku mapeto | Female | |
Nduna yowona za Mphamvu ya Magetsi ndi Migodi, a Newton Kambala, a Chris Chaima Banda omwe m’modzi mwa alangizi, a Chris Chaima Banda omwe m’modzi mwa alangizi mwa President Lazarus Chakwera | Nduna yowona za Mphamvu ya Magetsi ndi Migodi, a Nyutoni Kambala, a khilisi Chaima Banda omwe m’modzi mwa alangizi, a khilisi Chaima Banda omwe m’modzi mwa alangizi mwa pulezidenti lazalasi Chakwera | Female | |
komanso President wa chipani cha Alliance for Democracy (AFORD) a Enock Cha, a enock chakufwa Chihana usiku wathawu agona m'chitokosi cha apolisi ku Lilongwe | komanso pulezidenti wa chipani cha alayansi fo demokilase (AFODI) a inoki Cha, a inoki chakufwa Chihana usiku wathawu agona m'chitokosi cha apolisi ku Lilongwe | Female | |
kusatira kumangidwa kwawo ndi bungwe lothana ndi ziphuphu komanso katangale la ACB pa nkhani za katangale | kusatira kumangidwa kwawo ndi bungwe lothana ndi ziphuphu komanso katangale la esibi pa nkhani za katangale | Female | |
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI), mawa la Chitatu liyamba m’bindikiro ku nyumba ya malamulo | Bungwe lomenyera ufulu wa anthu la senta fo demokilase andi ikonomiki divelopumenti inishetivisi (SIDEDI), mawa la Chitatu liyamba m’bindikiro ku nyumba ya malamulo | Female | |
pofuna kuwumiliza kalariki wa nyumbayi Fiona Kalemba, sipikala Gotani Hara komanso Nduna ya za m’dziko a Richard Chimwendo Banda kuti afotokoze bwino | pofuna kuwumiliza kalariki wa nyumbayi Fiona Kalemba, sipikala Gotani Hara komanso Nduna ya za m’dziko a litchadi Chimwendo Banda kuti afotokoze bwino | Female | |
paza momwe bilu yopempha ngongole ku maiko a kunja inazembetsedwera kupita ku nyumba ya malamulo phungu asanayikambilane | paza momwe bilu yopempha ngongole ku maiko a kunja inazembetsedwera kupita ku nyumba ya malamulo phungu asanayikambilane | Female | |
Bambo wina wa zaka 41 zakubadwa m’boma la Mangochi wazipha pozimangalira pothawa mkwiyo wa anthu atamupezelera akugwilira mwana wake omupeza wa zaka 8 zakubadwa | Bambo wina wa zaka fotewani zakubadwa m’boma la Mangochi wazipha pozimangalira pothawa mkwiyo wa anthu atamupezelera akugwilira mwana wake omupeza wa zaka eiti zakubadwa | Female | |
Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali, a Amina Tepani Daudi , watsimikiza za nkhani-yi pomwe wati mkuluyu amadziwika ndi dzina loti Kasusu Lepha | Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali, a Amina Tepani Daudi , watsimikiza za nkhaniyi pomwe wati mkuluyu amadziwika ndi dzina loti Kasusu Lepha | Female | |
Dziko lino akuti ligwiritsa ntchito ndalama pafupifupi K4 billion pa msonkhano wa atsogoleri a maiko a m’bungwe la SADC omwe uchitike m’dziko muno kuyambira lero lolemba mpaka pa 19 August | Dziko lino akuti ligwiritsa ntchito ndalama pafupifupi folo biliyoni kwacha pa msonkhano wa atsogoleri a maiko a m’bungwe la SADIKI omwe uchitike m’dziko muno kuyambira lero lolemba mpaka pa Naintini ogasiti | Female | |
Nduna yoona za ubale wa dziko lino ndi maiko ena, Eisenhower Mkaka ndi yomwe yalengeza izi pa msonkhano wa atolankhani omwe inachititsa mu mzinda wa Lilongwe pa modzi pamodzi ndi nduna ya zofalitsa nkhani, Gospel Kazako | Nduna yoona za ubale wa dziko lino ndi maiko ena, eseni huwa Mkaka ndi yomwe yalengeza izi pa msonkhano wa atolankhani omwe inachititsa mu mzinda wa Lilongwe pa modzi pamodzi ndi nduna ya zofalitsa nkhani, Gosipelo Kazako | Female | |
M’busa Martin Thom yemwe kufikira lero lachiwiri anali mlingizi wa pa padera wa President Lazarus Chakwera watulutsidwa pa bail ya polisi | M’busa Martin Thomu yemwe kufikira lero lachiwiri anali mlingizi wa pa padera wa Pulezidenti Lazalasi Chakwera watulutsidwa pa belo ya polisi | Female | |
atakhala kwa maola ochepa chabe mchitokosi kutsatira kumangidwa kwake pamodzi ndi, pamodzi ndi m’modzi wa akuluakulu ku unduna wa za chuma, Nations Msowoya | atakhala kwa maola ochepa chabe mchitokosi kutsatira kumangidwa kwake pamodzi ndi, pamodzi ndi m’modzi wa akuluakulu ku unduna wa za chuma, Neshonzi Msowoya | Female | |
A Thom ndi a Msowoya anamangidwa powaganizira kuti akukhudzidwa ndi kuzembetsedwa kwa kalata zopemphela ngongole ya boma ku maiko akunja | A Thomu ndi a Msowoya anamangidwa powaganizira kuti akukhudzidwa ndi kuzembetsedwa kwa kalata zopemphela ngongole ya boma ku maiko akunja | Female | |
Zomwe zinakapelekedwa ku nyumba ya malamulo pa mkumano omwe wangothawu koma boma lisakudziwa | Zomwe zinakapelekedwa ku nyumba ya malamulo pa mkumano omwe wangothawu koma boma lisakudziwa | Female | |
Lawyer yemwe akuimira abusa a Thom, Sylvester Ayuba James ndi yemwe watitsimikizira kuti mkuluyu watulutsidwa pa bail ya polisi ndipo ali ndi milandu inayi yomwe akuyenera kuyankha | Loyar yemwe akuimira abusa a Thomu, Silivesita Ayuba Jemusi ndi yemwe watitsimikizira kuti mkuluyu watulutsidwa pa belo ya polisi ndipo ali ndi milandu inayi yomwe akuyenera kuyankha | Female | |
Milandu malingana ndi Ayuba James, ndi kugwiritsa ntchito ofesi ya boma molakwika, kukonza upo ofuna kubera boma, kulemba kalata za chinyengo popanda chilolezo mwa ina | Milandu malingana ndi Ayuba Jemusi, ndi kugwiritsa ntchito ofesi ya boma molakwika, kukonza upo ofuna kubera boma, kulemba kalata za chinyengo popanda chilolezo mwa ina | Female | |
Pakadali pano, lawyer-yu wati mbali yoganizilidwa ndi yokonzedwa kuonetsa bwalo la milandu kuti boma likungowanamizira pa nkhani zonse zomwe lawatsegulira | Pakadali pano, loyayu wati mbali yoganizilidwa ndi yokonzedwa kuonetsa bwalo la milandu kuti boma likungowanamizira pa nkhani zonse zomwe lawatsegulira | Female | |
Atangomangidwa a Thom, President Lazarus Chakwera anachotsa a Thom pa udindo wawo ngati mlangizi wake wapadera ngakhale Othandizira Presidentiyu, Sean Kampondeni anati a Chakwera samadziwa za nkhaniyi pa chiyambi | Atangomangidwa a Thomu, Pulezidenti Lazalasi Chakwera anachotsa a Thomu pa udindo wawo ngati mlangizi wake wapadera ngakhale Othandizira Pulezidentiyu, Shoni Kampondeni anati a Chakwera samadziwa za nkhaniyi pa chiyambi | Female | |
Pali kutsutsana mau pakati pa Mneneri wa President Wa dziko lino Brian Banda ndi bwana wawo yemwenso ndi m’thandizi wa mkulu wa President | Pali kutsutsana mau pakati pa Mneneri wa Pulezidenti Wa dziko lino Bulayani Banda ndi bwana wawo yemwenso ndi m’thandizi wa mkulu wa Pulezidenti | Female | |
a Sean Kampondeni pa momwe ziliri mu office ya oyankhulira President Lazarus Chakwera pamene zikumveka kuti a Brian Banda awachotsa pa udindowu ndipo pasankhidwa munthu wina m’malo mwawo | a Sean Kampondeni pa momwe ziliri mu ofesi ya oyankhulira Pulezidenti Lazalasi Chakwera pamene zikumveka kuti a Bulayani Banda awachotsa pa udindowu ndipo pasankhidwa munthu wina m’malo mwawo | Female | |
A Brian Banda awuza atolankhani a Nation Newspaper kuti iwo asiya ntchitoyo chifukwa akupita ku school ku China, komwe akakhaleko kwa miyezi inayi | A Brian Banda awuza atolankhani a nashoni nyuzi pepa kuti iwo asiya ntchitoyo chifukwa akupita ku sukulu ku tchaina, komwe akakhaleko kwa miyezi inayi | Female | |
Pamene a Sean Kampondeni atafunsidwa za nkhani ati zoti papezeka munthu wina olomwa mmalo mwa a Banda ndizoona koma zoti a Banda asiya okha ntchito mene akunenela sakuziziwa | Pamene a Shoni Kampondeni atafunsidwa za nkhani ati zoti papezeka munthu wina olomwa mmalo mwa a Banda ndizoona koma zoti a Banda asiya okha ntchito mene akunenela sakuziziwa | Female | |
Atafunsindwa ndi atolankhani za munthu amene wasankhidwa kulowa mmalo mwa Brian Banda, a Kampondeni anakana kuntchula poneneka kuti President Lazarus Chakwera atchula yekha munthu amene amusankha akakonzeka | Atafunsindwa ndi atolankhani za munthu amene wasankhidwa kulowa mmalo mwa Bulayani Banda, a Kampondeni anakana kuntchula poneneka kuti Pulezidenti Lazalasi Chakwera atchula yekha munthu amene amusankha akakonzeka | Female | |
Gule wa Mkulu ali m’chitokosi cha apolisi m’boma la Mchinji pomuganizira kuti wagwilira mayi wina m’mudzi mwa Nyongani m’dera la mfumu yaikulu Mavwere m’bomali | Gule wa Mkulu ali m’chitokosi cha apolisi m’boma la Mchinji pomuganizira kuti wagwilira mayi wina m’mudzi mwa Nyongani m’dera la mfumu yaikulu Mavwere m’bomali | Female | |
Mkulu wa polisi ya Mchinji, Charles James Mpezeni watsimikiza za kumangidwa kwa chirombocho chomwe chikudziwika ndi dzina loti Moyenda Jephter | Mkulu wa polisi ya Mchinji, tchalosi Jemusi Mpezeni watsimikiza za kumangidwa kwa chirombocho chomwe chikudziwika ndi dzina loti Moyenda Jafita | Female | |
Malingana ndi a Mpezeni, Gule Wa Mkulu yu anagwilira mayiyu ngati chilango ati kaamba koti sanapite ku mwambo wa chiliza omwe umachitika m’mudzimo | Malingana ndi a Mpezeni, Gule Wa Mkulu yu anagwilira mayiyu ngati chilango ati kaamba koti sanapite ku mwambo wa chiliza omwe umachitika m’mudzimo | Female | |
Moyenda Japhter akuyembekezeka kukawonekera ku bwalo la Milandu komwe akayakhe mlandu ogwilira | Moyenda Jafita akuyembekezeka kukawonekera ku bwalo la Milandu komwe akayakhe mlandu ogwilira | Female | |
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Center for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) lauza President Lazarus Chakwera kuti aimitse ulendo wake opita ku United Kingdom | Bungwe lomenyera ufulu wa anthu la senta fo demokilase andi ikonomiki divelopumenti inishetivisi (SIDEDI) lauza Pulezidenti Lazalasi Chakwera kuti aimitse ulendo wake opita ku Yunaitedi king’idomu | Female | |
ponena kuti zolinga za ulendowu sizipindulira dziko. A Chakwera pamodzi ndi anthu ena pafupifupi khumi apita ku UK mawa lamulungu | ponena kuti zolinga za ulendowu sizipindulira dziko. A Chakwera pamodzi ndi anthu ena pafupifupi khumi apita ku yukeyi mawa lamulungu | Female | |
kukakhala nawo pa mkumano wa za maphunziro omwe nduna yaikulu ya dzikolo, Boris Johnson komanso mtsogoleri wa dziko la Kenya, Uhuru Kenyata akonza | kukakhala nawo pa mkumano wa za maphunziro omwe nduna yaikulu ya dzikolo, Borisi Jonisonin komanso mtsogoleri wa dziko la Kenya, Uhuru Kenyata akonza | Female | |
Koma malingana ndi bungwe la CDEDI kudzera mchikalata chomwe latulutsa, pali umboni kuti kupatula mkumanoWu, palinso umboni oti a Chakwera ukakhala nawo pa mwambo wa ukwati wina ku UK ko | Koma malingana ndi bungwe la SIDEDI kudzera mchikalata chomwe latulutsa, pali umboni kuti kupatula mkumanowu, palinso umboni oti a Chakwera ukakhala nawo pa mwambo wa ukwati wina ku UK ko | Female | |
Mtsogoleri wa bungweli, Sylvester Namiwa wati ulendowu sulephereka iwo amema anthu kuti akasonkhane ku bwalo la ndege lomwe mtsogoleriyu akanyamukire pofuna kuti apite nawo limodzi | Mtsogoleri wa bungweli, silivesita Namiwa wati ulendowu sulephereka iwo amema anthu kuti akasonkhane ku bwalo la ndege lomwe mtsogoleriyu akanyamukire pofuna kuti apite nawo limodzi | Female | |
Bungweli ladzudzulanso ganizo la President Chakwera lotenga mwana wawo Violet komanso achibale ena ngati nthumwi pa ulendowu. Pakadali pano akuluakulu ofalitsa nkhani ku nyumba ya boma sanayankhulepo kanthu pa nkhaniyi | Bungweli ladzudzulanso ganizo la pulezidenti Chakwera lotenga mwana wawo Vayoleti komanso achibale ena ngati nthumwi pa ulendowu. Pakadali pano akuluakulu ofalitsa nkhani ku nyumba ya boma sanayankhulepo kanthu pa nkhaniyi | Female | |
Bambo wa zaka 46, Yokoniya Phiri wa m’boma la Kasungu yemwe amafuna kuti mkazi wake asiye business yofulula mowa wapezeka atazimangilira ku denga la mkati mwa nyumba yake | Bambo wa zaka fote sikisi, Yokoniya Phiri wa m’boma la Kasungu yemwe amafuna kuti mkazi wake asiye bizinezi yofulula mowa wapezeka atazimangilira ku denga la mkati mwa nyumba yake | Female | |
Wachiwiri kwa mneneri wapolisi ku Kasungu, Miracle Mkozi watsimikiza izi ponena kuti zachitika patangopita masiku ochepa, malemuyu atakangana ndi mkazi wake pa nkhani ya mowayi | Wachiwiri kwa mneneri wapolisi ku Kasungu, Milako Mkozi watsimikiza izi ponena kuti zachitika patangopita masiku ochepa, malemuyu atakangana ndi mkazi wake pa nkhani ya mowayi | Female | |
Malingana ndi Mkozi, mkaziyu anakana kumvera langizoli zomwe linautsa mkangano ndipo Patapita masiku ochepa ndi pomwe wapezeka akulendewera ku denga koma atafa | Malingana ndi Mkozi, mkaziyu anakana kumvera langizoli zomwe linautsa mkangano ndipo Patapita masiku ochepa ndi pomwe wapezeka akulendewera ku denga koma atafa | Female | |
Apolisi ati akukhulupilira kuti mkuluyu wachita kuzimangilira pa mbuyo pa mkanganowu. Malemu Yokoniya Phiri anali wa m’mudzi mwa Kaponda mfumu yaikulu Kaluluma ku Kasungu komweko | Apolisi ati akukhulupilira kuti mkuluyu wachita kuzimangilira pa mbuyo pa mkanganowu. Malemu Yokoniya Phiri anali wa m’mudzi mwa Kaponda mfumu yaikulu Kaluluma ku Kasungu komweko | Female | |
Williams Kajoloweka Kaponda yemwe ndi wapolisi pa polisi yaing’ono ya Ndonda wapereka thandizo la ma uniform kwa ophunzira khumi ndi atatu (13) a pa sukuku ya Primary ya Thithimira | Wiliyamuzi Kajoloweka Kaponda yemwe ndi wapolisi pa polisi yaing’ono ya Ndonda wapereka thandizo la ma yunifomu kwa ophunzira khumi ndi atatu (fetini) a pa sukuku ya Pulaimale ya Thithimira | Female | |
Malingana ndi Kaponda, wagwiritsa ntchito ndalama zomwe amapeza pa ntchito yake ngati wapolisi. Iye wati wachita izi chifukwa nayenso anathandizidwapo ndi anthu ena kuti afike pomwe ali pakadali pano | Malingana ndi Kaponda, wagwiritsa ntchito ndalama zomwe amapeza pa ntchito yake ngati wapolisi. Iye wati wachita izi chifukwa nayenso anathandizidwapo ndi anthu ena kuti afike pomwe ali pakadali pano | Female | |
M’mbuyomu, a Kaponda anasamusidwa pa polisi ya Nkhotakota komwe amagwira ntchito ngati mneneri wapolisiyi ponena kuti anasowa mwambo | M’mbuyomu, a Kaponda anasamusidwa pa polisi ya Nkhotakota komwe amagwira ntchito ngati mneneri wapolisiyi ponena kuti anasowa mwambo | Female | |
atalemba pa tsamba lawo la Facebook zokumbutsa lonjezo la President Chakwera kuti samazaimitsa apolisi mu mseu pomwe akufuna kudutsa | atalemba pa tsamba lawo la fesibuku zokumbutsa lonjezo la pulezidenti Chakwera kuti samazaimitsa apolisi mu mseu pomwe akufuna kudutsa | Female | |
Kupatula kupereka ma yunifolomu wa, mkuluyu waperekanso zolembera komanso makope kwa ophunzirawa | Kupatula kupereka ma yunifolomuwa, mkuluyu waperekanso zolembera komanso makope kwa ophunzirawa | Female | |
Bwalo la milandu mu mzinda wa Mzuzu lapeza yemwe anali mkulu wa polisi yaing’ono ya Nthalire ku Chitipa, Ben Mwaliwa ndi mlandu oti ayankhe | Bwalo la milandu mu mzinda wa Mzuzu lapeza yemwe anali mkulu wa polisi yaing’ono ya Nthalire ku Chitipa, Beni Mwaliwa ndi mlandu oti ayankhe | Female | |
anthu ena atamuneneza ku bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu la ACB kuti analandira chiphuphu kuti atulutse munthu wina mchitokosi koma mosasata ndondomeko | anthu ena atamuneneza ku bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu la esibi kuti analandira chiphuphu kuti atulutse munthu wina mchitokosi koma mosasata ndondomeko | Female | |
Mwaliwa anamangidwa ndi bungweli ndipo malingana ndi mneneri wa ACB, Egritta Ndala, mkuluyu ali ndi milandu itatu yoti ayankhe | Mwaliwa anamangidwa ndi bungweli ndipo malingana ndi mneneri wa esibi, Egirita Ndala, mkuluyu ali ndi milandu itatu yoti ayankhe | Female | |
Mai Ndala ati milanduyi ndi kuphatikizapo kugwiritsa ntchito ofesi molakakwika komanso ina iwiri ya katangale | Mai Ndala ati milanduyi ndi kuphatikizapo kugwiritsa ntchito ofesi molakakwika komanso ina iwiri ya katangale | Female | |
Mlanduwu upitilire pa 11 August chaka chino omwe Mwaliwa akakane kapena kuvomera milanduyi | Mlanduwu upitilire pa leveni ogasiti chaka chino omwe Mwaliwa akakane kapena kuvomera milanduyi | Female | |
Apolisi m’boma la Dedza atsekera mchitokosi mwini wake wa sukulu ina ya mkombaphala m’bomalo pomuganizira kuti wagwilira mwana wa zaka zisanu ndi chimodzi (6) yemwe amaphunzira pa sukuluyi | Apolisi m’boma la Dedza atsekera mchitokosi mwini wake wa sukulu ina ya mkombaphala m’bomalo pomuganizira kuti wagwilira mwana wa zaka zisanu ndi chimodzi (sikisi) yemwe amaphunzira pa sukuluyi | Female | |
Malipoti akuti oganizilidwayu yemwe ndi Austin Chilanga anapereka ntchito ya mkalasi kwa anawa ndipo onse Atamaliza anawauza kuti azipita ku nyumba koma m’modzi yekha atsale | Malipoti akuti oganizilidwayu yemwe ndi ositini Chilanga anapereka ntchito ya mkalasi kwa anawa ndipo onse Atamaliza anawauza kuti azipita ku nyumba koma m’modzi yekha atsale | Female | |
Malingana ndi apolisi, apa mkuluyu anauza mwanayu kuti agone kenako anamugwililira ndipo anamugulira kamba ngati chitseka pakamwa koma patangotha masiku awiri, mwanayu anayamba Kuvutika poyenda | Malingana ndi apolisi, apa mkuluyu anauza mwanayu kuti agone kenako anamugwililira ndipo anamugulira kamba ngati chitseka pakamwa koma patangotha masiku awiri, mwanayu anayamba Kuvutika poyenda | Female | |
Makolo ake atamufunsa ndi pomwe anaulula zomwe Chilanga anamuchita ndipo Makolowa anakamuneneza mkuluyu ku polisi ngakhale anali atathawa kufikira lolemba lapitali pomwe amammanga | Makolo ake atamufunsa ndi pomwe anaulula zomwe Chilanga anamuchita ndipo Makolowa anakamuneneza mkuluyu ku polisi ngakhale anali atathawa kufikira lolemba lapitali pomwe amammanga | Female | |
Poyankhapo chilanga anati anachita izi kaamba ka satana yemwe anamunamiza kuti atero | Poyankhapo chilanga anati anachita izi kaamba ka satana yemwe anamunamiza kuti atero | Female | |
Komiti ya nyumba ya malamulo yoona za thumba la chitukuko cha m’madera a aphungu la CDF yati ikukonza zokumana ndi mabungwe onse | Komiti ya nyumba ya malamulo yoona za thumba la chitukuko cha m’madera a aphungu la sidiefu yati ikukonza zokumana ndi mabungwe onse | Female | |
opopa ndi kugulitsa madzi m’dziko ndi cholinga chozakambirana zambiri zokhuza mijigo yomwe amakumba m’matawuni | opopa ndi kugulitsa madzi m’dziko ndi cholinga chozakambirana zambiri zokhuza mijigo yomwe amakumba m’matawuni | Female | |
Malingana ndi wa pa mpando wa komitiyi, Ralph Joma komiti yawo inachita kale kafukufuku komanso kulemba lipoti pa momwe mijigoyi imagwilira ntchito m’mizinda ndi matawuni | Malingana ndi wa pa mpando wa komitiyi, Rafu Joma komiti yawo inachita kale kafukufuku komanso kulemba lipoti pa momwe mijigoyi imagwilira ntchito m’mizinda ndi matawuni | Female | |
Malingana ndi Joma, zotsatira za lipotili azipereka pa mkumano omwe achititsewu ndipo azachitanso kauniuni pa nkhawa zomwe zimakhalapo | Malingana ndi Joma, zotsatira za lipotili azipereka pa mkumano omwe achititsewu ndipo azachitanso kauniuni pa nkhawa zomwe zimakhalapo | Female | |
Mbali zosiyanasiyana zakhala zikukhala zikuonetsa kusakondwa pa ukhondo komanso kutetezeka kwa madzi omwe mijigo ya m’matawuni imapereka kwa anthu ngakhale kuti mijigoyi imathandiza madzi a pa mpopi akasiya | Mbali zosiyanasiyana zakhala zikukhala zikuonetsa kusakondwa pa ukhondo komanso kutetezeka kwa madzi omwe mijigo ya m’matawuni imapereka kwa anthu ngakhale kuti mijigoyi imathandiza madzi a pa mpopi akasiya | Female | |
Kutsatira kukula kwa ziwawa zomwe anthu m’dziko la South Africa akuchita pofuna kuti mtsogoleri wakale wa dzikolo atuluke ku ndende, boma latumiza asilikali m’mizinda yonse kukathandiza apolisi pa ntchito yokhazikitsa bata | Kutsatira kukula kwa ziwawa zomwe anthu m’dziko la Saufi afilika akuchita pofuna kuti mtsogoleri wakale wa dzikolo atuluke ku ndende, boma latumiza asilikali m’mizinda yonse kukathandiza apolisi pa ntchito yokhazikitsa bata | Female | |
Mwa zina, anthuwa aphwanya kale malo ogulitsira malonda osiyanasiyana mu mzinda wa Durban ndi mmizinda ina ndipo malingana ndi nyumba yofalitsa nkhani ya boma ya SABC, katundu wa ndalama za nkhaninkhani waonongedwa kale | Mwa zina, anthuwa aphwanya kale malo ogulitsira malonda osiyanasiyana mu mzinda wa Dabeni ndi mmizinda ina ndipo malingana ndi nyumba yofalitsa nkhani ya boma ya sabiki, katundu wa ndalama za nkhaninkhani waonongedwa kale | Female | |
Nawo malipoti a nyuzipepala ya Eyewitness News akuti bata linasokonekeranso ku dera la Kwazulu Nata dzulo lolemba | Nawo malipoti a nyuzipepala ya aye witinesi nyuzi akuti bata linasokonekeranso ku dera la Kwazulu Nata dzulo lolemba | Female | |
zomwe zinachititsa kuti malo operekera Katemera wolimbana ndi mliri wa COVID-19 atsekedwe mwachangu | zomwe zinachititsa kuti malo operekera Katemera wolimbana ndi mliri wa Kovidi-naintini atsekedwe mwachangu | Female | |
Apolisi ku Nkhotakota atsekera mchitokosi mnyamata wa zaka 20 zakubadwa pomuganizira kuti watentha nyumba ya munthu wina, atayambana ndi mwana wake ku mowa | Apolisi ku Nkhotakota atsekera mchitokosi mnyamata wa zaka twente zakubadwa pomuganizira kuti watentha nyumba ya munthu wina, atayambana ndi mwana wake ku mowa | Female | |
Mneneri wa polisi ya Nkhotakota, Paul Malimwe watiuza kuti opalamula-yu ndi Lufeyo Osten ndipo anapalamula mlanduwu masana a pa 9 July | Mneneri wa polisi ya Nkhotakota, Po Malimwe watiuza kuti opalamulayu ndi Lufeyo Ositeni ndipo anapalamula mlanduwu masana a pa naini julayi | Female | |
pa mbuyo pa ndeu yomwe inabuka pa malo ena omwera mowa ndi mwana wa mwini nyumbayu. Malingana ndi Malimwe, katundu wa ndalama pafupifupi K108 thousand waonongeka kutsatira kuotchedwa kwa nyumbayu | pa mbuyo pa ndeu yomwe inabuka pa malo ena omwera mowa ndi mwana wa mwini nyumbayu. Malingana ndi Malimwe, katundu wa ndalama pafupifupi wani handiledi andi eiti sauzande kwacha waonongeka kutsatira kuotchedwa kwa nyumbayu | Female | |
Osten yemwe ndi wa pa mudzi pa Kasakula, mfumu yaikulu Mwadzama m’bomalo, akaonekera ku bwalo la milandu posachedwapa | Ositeni yemwe ndi wa pa mudzi pa Kasakula, mfumu yaikulu Mwadzama m’bomalo, akaonekera ku bwalo la milandu posachedwapa | Female | |
kukayankha mlandu ootcha nyumba zomwe ndi zosemphana ndi gawo 337 la malamulo a milandu | kukayankha mlandu ootcha nyumba zomwe ndi zosemphana ndi gawo filifili seveni la malamulo a milandu | Female | |
Nzika yina ya m’dziko la china ili m’manja mwa apolisi m’boma la Nkhata Bay poyiganizira kuti yakhala ikuchitira khanza ogwira ntchito a chizimayi po mawagwira malo obisika zomwe ndi zotsutsana ndi malamulo a dziko lino | Nzika yina ya m’dziko la china ili m’manja mwa apolisi m’boma la Nkhatabe poyiganizira kuti yakhala ikuchitira khanza ogwira ntchito a chizimayi po mawagwira malo obisika zomwe ndi zotsutsana ndi malamulo a dziko lino | Female | |
Mneneri wa apolisi ku Nkhatabay, Kondwani James wati oganizilidwayu Chen Shilliang amagwira ntchito pa kampani yina ya m’dziko la China yomwe inapatsidwa ntchito yokumba mijigo m’bomali | Mneneri wa apolisi ku Nkhatabe, Kondwani Jemusi wati oganizilidwayu Tcheni Shiliyang’i amagwira ntchito pa kampani yina ya m’dziko la China yomwe inapatsidwa ntchito yokumba mijigo m’bomali | Female | |
A polisi m’boma la Nkhata Bay amanga mayi wina wa zaka 29 zakubadwa pomuganizira kuti anazijambura kanema olawula ndikumagawa pa matsamba a mchezo apa internet | A polisi m’boma la Nkhatabe amanga mayi wina wa zaka twente naini zakubadwa pomuganizira kuti anazijambura kanema olawula ndikumagawa pa matsamba a mchezo apa intaneti | Female | |
Mneneri wa apolisi m’boma-li, Kondwani James watsimikiza za nkhani-yi ndipo wati mayi ndi wa m’mudzi mwa Kamphalo m’dera la mfumu yaikulu Timbiri m’boma la Nkhata Bay | Mneneri wa apolisi m’bomali, Kondwani Jemusi watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati mayi ndi wa m’mudzi mwa Kamphalo m’dera la mfumu yaikulu Timbiri m’boma la Nkhatabe | Female | |
Musayiphonye nkhani-yi komanso nkhani zina zambiri mu nkhani za M'mitekete pa Ndirande FM, 95.9Mhz nthawi ya 9 Koloko m'mawa uno | Musayiphonye nkhaniyi komanso nkhani zina zambiri mu nkhani za M'mitekete pa Ndirande rfuemu, nainte faifi pointi naini megahedzi nthawi ya naini Koloko m'mawa uno | Female | |
Lero ku m'mawaku anthu mu mzinda wa Blantyre anali odabwa kuona chithunzi Cha munthu wina wa mai ali pa Chikwangwani ngati imodzi mwa njira yosonyeza mafuno abwino pa tsiku lake lobadwa | Lero ku m'mawaku anthu mu mzinda wa Bulantaya anali odabwa kuona chithunzi Cha munthu wina wa mai ali pa Chikwangwani ngati imodzi mwa njira yosonyeza mafuno abwino pa tsiku lake lobadwa | Female | |
Chikwangwanichi chomwenso Ndirande FM yaona itayendera malo omwe chili, chilinso ndi mau omwe akuonetsa chikondi chozama chomwe mwamunayi ali nacho pa mkazi wake | Chikwangwanichi chomwenso Ndirande efuemu yaona itayendera malo omwe chili, chilinso ndi mau omwe akuonetsa chikondi chozama chomwe mwamunayi ali nacho pa mkazi wake | Female | |
Anthu ochuluka akhala akukhamukira pa malo-wa pomwe ndi pafupi ndi banki yaikulu ya FDH kuti azazionere okha ndipo ena anagwiritsa ntchito lamya zawo za mmanja kujambula Chikwangwanichi ndikutumizira amnzawo | Anthu ochuluka akhala akukhamukira pa malowa pomwe ndi pafupi ndi banki yaikulu ya efudietchi kuti azazionere okha ndipo ena anagwiritsa ntchito lamya zawo za mmanja kujambula Chikwangwanichi ndikutumizira amnzawo | Female | |
Pakadali pano, izi zausa mtsutso pa masamba a mchezo pomwe abambo ambiri ati izi zichititsa kuti akhale pa mpanimpani ochita zinthu zoposera apa ngati mbali imodzi yoonetsa chikondi kwa okondedwa awo | Pakadali pano, izi zausa mtsutso pa masamba a mchezo pomwe abambo ambiri ati izi zichititsa kuti akhale pa mpanimpani ochita zinthu zoposera apa ngati mbali imodzi yoonetsa chikondi kwa okondedwa awo | Female | |
Komatu amai ambiri ayamikira mwamuna yemwe waika mkazi pa chikwangwaniyi ponena kuti ichi Ndi chizindikiro cha chikondi chenicheni | Komatu amai ambiri ayamikira mwamuna yemwe waika mkazi pa chikwangwaniyi ponena kuti ichi Ndi chizindikiro cha chikondi chenicheni | Female | |
Izitu zachitika pomwe lamulungu lapitali linali tsiku lokumbukira abambo pa dziko lonse la pansi | Izitu zachitika pomwe lamulungu lapitali linali tsiku lokumbukira abambo pa dziko lonse la pansi | Female | |
Apolisi m’boma la Dedza awalangiza kuti azitenga dandaulo lililonse kuchokera kwa anthu ngati lofunika posayang’anira kuchepa kwa dandaulolo kapena mphanvu za Munthu yemwe akupereka dandaulo | Apolisi m’boma la Dedza awalangiza kuti azitenga dandaulo lililonse kuchokera kwa anthu ngati lofunika posayang’anira kuchepa kwa dandaulolo kapena mphanvu za Munthu yemwe akupereka dandaulo | Female | |
Mkulu wa apolisi ku Dedza Mwizamose Nyoni ndi yemwe wapereka langizoli ponena kuti aliyense ndi ofunika choncho ufulu wake opeza chilungamo ukuyenera kulemekezedwa | Mkulu wa apolisi ku Dedza Mwizamose Nyoni ndi yemwe wapereka langizoli ponena kuti aliyense ndi ofunika choncho ufulu wake opeza chilungamo ukuyenera kulemekezedwa | Female | |
A Nyoni ati kulemekeza madando a anthu maka a madera a ku mudzi kuli ndi kuthekera kothandizanso kuti ubale wa apolisi ndi anthu a m’dera uzikhala wabwino | A Nyoni ati kulemekeza madando a anthu maka a madera a ku mudzi kuli ndi kuthekera kothandizanso kuti ubale wa apolisi ndi anthu a m’dera uzikhala wabwino | Female | |
Mkulu wa apolisi ku a ku Dedzayu amayankhula izi pomwe amayendera mapolisi osiyana-siyana a m’bomali pofuna kuona momwe akugwilira ntchito | Mkulu wa apolisi ku a ku Dedzayu amayankhula izi pomwe amayendera mapolisi osiyanasiyana a m’bomali pofuna kuona momwe akugwilira ntchito | Female | |
M’mawu ake, m’modzi mwa apolisi omwe alandira nawo upangiriwu, Alfred Kaliba anati apolisi amva langizoli ndipo asintha kachitidwe ka zinthu | M’mawu ake, m’modzi mwa apolisi omwe alandira nawo upangiriwu, Alafuledi Kaliba anati apolisi amva langizoli ndipo asintha kachitidwe ka zinthu | Female | |
Achinyamata mu mzinda wa Mzuzu ati atopa ndi kudikilira kuti boma la Mgwirizano wa Tonse tikwaniritse lonjezo lomanga malo ochitirapo ntchito zosiyanasiyana za achinyamata a Mzuzu Youth Center | Achinyamata mu mzinda wa Mzuzu ati atopa ndi kudikilira kuti boma la Mgwirizano wa Tonse tikwaniritse lonjezo lomanga malo ochitirapo ntchito zosiyanasiyana za achinyamata a Mzuzu yufi senta | Female | |
Anthu a m’mizinda ya Blantyre ndi Lilongwe omwe akuyenera kulandira katemera Wachiwiri wa COVID-19 pambuyo pa sabata khumi ndi ziwiri atalandira oyamba, akuyenera kudikira kwa ka nthawi asanatero | Anthu a m’mizinda ya Bulantaya ndi Lilongwe omwe akuyenera kulandira katemera Wachiwiri wa Kovidi-naintini pambuyo pa sabata khumi ndi ziwiri atalandira oyamba, akuyenera kudikira kwa ka nthawi asanatero | Female | |
Izitu zili ndi chomwechi kutsatira kubwera poyera kwa maofesi ya zaumoyo m’mizindayi omwe ati katemera wa AstraZenicayu watha mmalo ake onse operekera | Izitu zili ndi chomwechi kutsatira kubwera poyera kwa maofesi ya zaumoyo m’mizindayi omwe ati katemera wa AsitiraZenikayu watha mmalo ake onse operekera | Female | |
Ofesi ya zaumoyo ku Blantyre mwa mkulu wake, Dr. Gift Kawalazira yati katemera wina akapezeka ilengeza | Ofesi ya zaumoyo ku Bulantaya mwa mkulu wake, Dokota Gifiti Kawalazira yati katemera wina akapezeka ilengeza | Female | |
Pamene ku Lilongwe, mkulu wa zaumoyo mu mzindawu, Dr. Alinafe Tambala wati anthu asadele nkhawa ngakhale nthawi yawo yolandira katemerayu itadusa | Pamene ku Lilongwe, mkulu wa zaumoyo mu mzindawu, Dokota Alinafe Tambala wati anthu asadele nkhawa ngakhale nthawi yawo yolandira katemerayu itadusa | Female | |
Izi zikhuzanso anthu ena omwe anali asanalandire katemerayu koma anali ndi malingaliro otero | Izi zikhuzanso anthu ena omwe anali asanalandire katemerayu koma anali ndi malingaliro otero | Female | |
Bambo wa zaka 40 zakubadwa George Kadzuwa amugamula kukhala ku ndende kwa zaka zitatu atapezeka olakwa pa mlandu ootcha nyumba ya mkazi wake wa kale m’boma la Nkhotakota | Bambo wa zaka fote zakubadwa Joji Kadzuwa amugamula kukhala ku ndende kwa zaka zitatu atapezeka olakwa pa mlandu ootcha nyumba ya mkazi wake wa kale m’boma la Nkhotakota | Female | |
Bwalo la milandu la Nkhunga First Grade Magistrate linamva mlandu wa mkuluyu kudzera mwa Oimira boma pa mlandu, Mickeas Chatsira yemwe anati Kadzuwa anachita za upanduzi usiku wa pa 23 April chaka chino | Bwalo la milandu la Nkhunga fesiti giledi majesitileti linamva mlandu wa mkuluyu kudzera mwa Oimira boma pa mlandu, Mikeyasi Chatsira yemwe anati Kadzuwa anachita za upanduzi usiku wa pa twente fili epulo chaka chino | Female | |
Malingana ndi Chatsira, mwini nyumbayi yemwe ndi mkazi wake wakale wa opalamulayu amagona cha ma 11 koloko usiku koma anazimumuka ndi utsi omwe unakuta chipinda chomwe anali ndipo atatuluka panja anazindikira kuti ndi moto | Malingana ndi Chatsira, mwini nyumbayi yemwe ndi mkazi wake wakale wa opalamulayu amagona cha ma leveni koloko usiku koma anazimumuka ndi utsi omwe unakuta chipinda chomwe anali ndipo atatuluka panja anazindikira kuti ndi moto | Female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.