audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Ma tsiku apitawo Board ya Mera inalengeza kuti yasankha a Henry Kachaje ngati mkulu wa bungweli
Ma tsiku apitawo Bodi ya Mera inalengeza kuti yasankha a Henele Kachaje ngati mkulu wa bungweli
Female
Nkhondo ya mawu yakula pakati pa m’busa Hastings Salanje wa mpingo wa God’s Chapel international komanso Prophet Austin Liabunya
Nkhondo ya mawu yakula pakati pa m’busa Hesiting’izi Salanje wa mpingo wa Godzi Ctchapelo intaneshono komanso Pulofeti Ositini Liyabunya
Female
wa utumiki wa Believers Gospel Embassy International, pa za yemwe ndi Mtumiki weni weni wa Mulungu
wa utumiki wa Bilivazi gosipelo embase intaneshono, pa za yemwe ndi Mtumiki weni weni wa Mulungu
Female
Mlembi wamkulu wa bungweli, Dorothy Nampota wati ophunzira omwe akukumana ndi mavuto pa nkhani ya ziphatso zawo akhalabe ndi mwai olemba mayeso poti MANEB yaika kale ndondomeko zowathandiza kutero
Mlembi wamkulu wa bungweli, Dolofe Nampota wati ophunzira omwe akukumana ndi mavuto pa nkhani ya ziphatso zawo akhalabe ndi mwai olemba mayeso poti Manebu yaika kale ndondomeko zowathandiza kutero
Female
Ndipo m'mau ake, nduna ya zamaphunziro, Agnes Nyalonje inafunira zabwino zonse ophunzira omwe akulemba mayesowa
Ndipo m'mau ake, nduna ya zamaphunziro, Aginesi Nyalonje inafunira zabwino zonse ophunzira omwe akulemba mayesowa
Female
Bwalo lalikulu la milandu mu mzinda wa Blantyre lachisanu likubwelera likuyembekezereka kuzapereka chigamulo chake pa nkhani yomwe bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu la ACB
Bwalo lalikulu la milandu mu mzinda wa Bulantaya lachisanu likubwelera likuyembekezereka kuzapereka chigamulo chake pa nkhani yomwe bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu la esibi
Female
likuganizira mpondamatiki Thomson Mpinganjira kuti amafuna kupereka ziphuphu kwa oweruza asanu omwe amanva mlandu wa chisankho cha mtsogoleri cha mu 2019
likuganizira mpondamatiki Thomusoni Mpinganjira kuti amafuna kupereka ziphuphu kwa oweruza asanu omwe amanva mlandu wa chisankho cha mtsogoleri cha mu twente naintini
Female
Malingana ndi kalata yomwe mlembi wamkulu ku High komanso Supreme Court, Gladys Gondwe wasainira, oweruza Dorothy DeGabrielle yemwe amanva nkhaniyi
Malingana ndi kalata yomwe mlembi wamkulu ku Hayi komanso Supulimu khoti, Giladesi Gondwe wasainira, oweruza Dolofe DeGabuliele yemwe amanva nkhaniyi
Female
akuyembekezereka kuzapereka chigamulochi nthawi ya 10 koloko m'mawa. Oweruzawa omwe amatsogozedwa ndi a Harley Potani anakamang'ala ku ACB
nkhaniyi akuyembekezereka kuzapereka chigamulochi nthawi ya teni koloko m'mawa. Oweruzawa omwe amatsogozedwa ndi a Hale Potani anakamang'ala ku esibi
Female
ponena kuti a Mpinganjira amafuna kupereka ziphuphu kuti bwalo la milandu lomwe pa nthawiyo linali la za malamulo, constitutional court mchingerezi, likondere imodzi mwa mbali zokhuzidwa pa mlanduwo
ponena kuti a Mpinganjira amafuna kupereka ziphuphu kuti bwalo la milandu lomwe pa nthawiyo linali la za malamulo, konsitichushono khoti mchingerezi, likondere imodzi mwa mbali zokhuzidwa pa mlanduwo
Female
Mlanduwu umakhuza mtsogoleri wakale wa dziko lino, Peter Mutharika ngati oyankhapo oyamba, bungwe la zisankho la Mec ngati oyankhapo achiwiri
Mlanduwu umakhuza mtsogoleri wakale wa dziko lino, Pita Mutharika ngati oyankhapo oyamba, bungwe la zisankho la Meki ngati oyankhapo achiwiri
Female
komanso a Saulos Chilima ngati odandaula oyamba ndi a Lazarus Chakwera ngati odaula achiwiri omwe amati chisankhocho chinali ndi zolakwika, pempho lomwe oweruzawa anagwirizana nalo
komanso a Saulosi Chilima ngati odandaula oyamba ndi a Lazalasi Chakwera ngati odaula achiwiri omwe amati chisankhocho chinali ndi zolakwika, pempho lomwe oweruzawa anagwirizana nalo
Female
Nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka mdziko muno ya Immigration yati lero itumiza kwawo mzika za dziko la Ethiopia zomwe zinalowa m'dziko muno mozembera malamulo
Nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka mdziko muno ya Imigileshoni yati lero itumiza kwawo mzika za dziko la Efiyopiya zomwe zinalowa m'dziko muno mozembera malamulo
Female
Mzikazi zomwe ndi zopitilira 100 zinagwidwa pakati pa miyezi ya November chaka chatha komanso March chaka chino
Mzikazi zomwe ndi zopitilira wani handiledi zinagwidwa pakati pa miyezi ya Novemba chaka chatha komanso Machi chaka chino
Female
Mneneri wa nthambi ya immigration mchigawo cha pakati, Martin Gongolo wati anthuwa azela pa bwalo la ndege Kamuzu International
Mneneri wa nthambi ya imigileshoni mchigawo cha pakati, Matini Gongolo wati anthuwa azela pa bwalo la ndege Kamuzu Intaneshono
Female
mothandizidwa ndi bungwe loona za anthu olowa ndi kutuluka m'maiko osiyanasiyana pa dziko lonse pa pansi ya Internation Organization on Migration
mothandizidwa ndi bungwe loona za anthu olowa ndi kutuluka m'maiko osiyanasiyana pa dziko lonse pa pansi ya intaneshono oganaizeshoni oni maigileshoni
Female
Bungwe la EDU FUND mogwilizana ndi gulu la anthu opalasa njinga mu mzinda wa Blantyre la Blantyre Cyclist Crew lero liri ndi ulendo opalasa njinga
Bungwe la ejufandi mogwilizana ndi gulu la anthu opalasa njinga mu mzinda wa Bulantaya la bulantaya saikilisiti khuluu lero liri ndi ulendo opalasa njinga
Female
omwe cholinga chake ndi kupeza ndalama zothandizira ophunzira osowa pa sukulu ya ukachenjede ya Malawi University of Business and Applied Sciences (MUBAS)
omwe cholinga chake ndi kupeza ndalama zothandizira ophunzira osowa pa sukulu ya ukachenjede ya Malawi yunivesite ofu bizinezi andi apulaidi sayansezi (MUBASI)
Female
Ulendowu wayambira pa sukulu ya MUBAS yomwe kale imadziwika kuti Polytechnic mu mzinda was Blantyre ndipo ukathera ku sukulu ya ukanjede ya University of Malawi (UNIMA)
Ulendowu wayambira pa sukulu ya MUBASI yomwe kale imadziwika kuti poletekiniki mu mzinda wa bulantaya ndipo ukathera ku sukulu ya ukanjede ya yunivesite ofu Malawi (YUNIMA)
Female
yomwe kale imadziwika kuti Chancellor College (Chanco) m'boma la Zomba. Bungwe la EDUFUND lati likukonza zotolera ndalama zopitilira K35 Million
yomwe kale imadziwika kuti Tchansala koleji (Tchanko) m'boma la Zomba. Bungwe la Ejufandi lati likukonza zotolera ndalama zopitilira fete faifi miliyonii kwacha
Female
zomwe zithandize ophunzira 75. Apolisi ku Mangochi apeza katundu wa ndalama pafupifupi K2.5 million yemwe akumuganizira kuti anachita kubedwa ndi anthu ena m'bomalo
zomwe zithandize ophunzira sevente faifi. Apolisi ku Mangochi apeza katundu wa ndalama pafupifupi thu pointi faifi miliyoni kwacka yemwe akumuganizira kuti anachita kubedwa ndi anthu ena m'bomalo
Female
Katunduyu wapezeka kutsatira chipikisheni chomwe apolisi anachita pambuyo pa malipoti oti mbava zakhala zikuthyola ndi kuba katundu m'malo osiyanasiyana
Katunduyu wapezeka kutsatira chipikisheni chomwe apolisi anachita pambuyo pa malipoti oti mbava zakhala zikuthyola ndi kuba katundu m'malo osiyanasiyana
Female
Malingana ndi malipoti, apolisi amanganso a James Amidu a zaka 29 komanso a Mussah Folopenzi a zaka 21
Malingana ndi malipoti, apolisi amanganso a Jemusi Amidu a zaka twente naini komanso a Musa Folopenzi a zaka twente wani
Female
ndipo akufunafuna anthu ena awiri omwe akuganizilidwa kuti ndi omwe anachita za upanduwu. Mneneri wa polisi ya Blantyre, Peter Mchiza
ndipo akufunafuna anthu ena awiri omwe akuganizilidwa kuti ndi omwe anachita za upanduwu. Mneneri wa polisi ya Bulantaya, Pita Mchiza
Female
wati anthu angapo amangidwa pambuyo pa zipolowe zomwe zinabuka mu mzinda wa Blantyre pomwe apolisi amathira utsi okhetsa msonzi
wati anthu angapo amangidwa pambuyo pa zipolowe zomwe zinabuka mu mzinda wa Bulantaya pomwe apolisi amathira utsi okhetsa msonzi
Female
pofuna kubalalitsa anthu ochita malonda mu mphepete mwa miseu mu mzindawu. Malingana ndi a Mchiza, apolisi anathira utsiwu pofuna kukhazikitsa bata
pofuna kubalalitsa anthu ochita malonda mu mphepete mwa miseu mu mzindawu. Malingana ndi a Mchiza, apolisi anathira utsiwu pofuna kukhazikitsa bata
Female
pomwe anthu ochita malondawa anayamba kugenda anthu a ku khonsolo ya mzinda wa Blantyre omwe anabwera kuzawachotsa m'malowa
pomwe anthu ochita malondawa anayamba kugenda anthu a ku khonsolo ya mzinda wa Bulantaya omwe anabwera kuzawachotsa m'malowa
Female
Wina mwa utsi omwe unaponyedwa pa Nandozi unakagwera mgalimoto yina yomwe imayenda, zinthu zomwe zinasokoneza mayendedwe
Wina mwa utsi omwe unaponyedwa pa Nandozi unakagwera mgalimoto yina yomwe imayenda, zinthu zomwe zinasokoneza mayendedwe
Female
ndipo dalaivala wa galimotoyi anakaomba galimoto ina yomwe inali itangoima. Koma a Mchiza ati pakadali pano apolisi sanalandire lipoti lililonse lokhuza ngoziyi
ndipo dalaivala wa galimotoyi anakaomba galimoto ina yomwe inali itangoima. Koma a Mchiza ati pakadali pano apolisi sanalandire lipoti lililonse lokhuza ngoziyi
Female
Apolisi mu mzinda wa Blantyre akugwiritsa ntchito utsi okhesa msonzi pofuna kubalalitsa anthu omwe amachita malonda mphepete mwa msewu
Apolisi mu mzinda wa Bulantaya akugwiritsa ntchito utsi okhesa msonzi pofuna kubalalitsa anthu omwe amachita malonda mphepete mwa msewu
Female
Mtolankhaní wathu Noel Mkwaila yemwe akuonerera izi zikuchitika watiuza kuti anthu ambiri akubanika ndi usiwu omwe akuuthira malo osiyanasiyana ochitira malondawa
Mtolankhaní wathu Nowelo Mkwaila yemwe akuonerera izi zikuchitika watiuza kuti anthu ambiri akubanika ndi usiwu omwe akuuthira malo osiyanasiyana ochitira malondawa
Female
Kampani ya Sunbird Hotel yabwerezanso kuuza ogwira ntchito ake kuti ali okakamizidwa kulandira Katemera oteteza ku mliri wa COVID-19
Kampani ya sanibewodi hotelo yabwerezanso kuuza ogwira ntchito ake kuti ali okakamizidwa kulandira Katemera oteteza ku mliri wa kovidi-naintini
Female
Malingana ndi kalata yomwe kampaniyi yalembera ogwira ntchito akewa yomwe ife taona, aliyense akuyenera akhale atalandira Katemerayu pofika loweruka pa 18 September chaka chino
Malingana ndi kalata yomwe kampaniyi yalembera ogwira ntchito akewa yomwe ife taona, aliyense akuyenera akhale atalandira Katemerayu pofika loweruka pa eitini sepitemba chaka chino
Female
konyozera izi sazaloledwa kugwira ntchito m’malo onse omwe Sunbird Hotel ili. Kalatayi yati yemwe azaonetse umboni oti walandira katemerayu
konyozera izi sazaloledwa kugwira ntchito m’malo onse omwe sani bewodi hotelo ili. Kalatayi yati yemwe azaonetse umboni oti walandira katemerayu
Female
kapena wakayezetsa COVID-19 ndipo wapezeka kuti alibe ndi yemwe azaloledwe kugwira ntchito
kapena wakayezetsa kovidi-naintini ndipo wapezeka kuti alibe ndi yemwe azaloledwe kugwira ntchito
Female
Sunbird Hotel inali imodzi mwa kampani zoyambilira kuuza ogwira ntchito ake kuti alandire Katemera ngati akufuna kugwira ntchito, ngakhale malamulo a dziko lino amati Katemera wa COVID-19 siokakamiza
sani bewodi hotelo inali imodzi mwa kampani zoyambilira kuuza ogwira ntchito ake kuti alandire Katemera ngati akufuna kugwira ntchito, ngakhale malamulo a dziko lino amati Katemera wa kovidi-naintini siwokakamiza
Female
Posachedwapa, bungwe la zisankho la Mec komanso kampani ya lamya za m’manja ya TNM ndi kampani zina, zauzanso ogwira ntchito ake kuti akuyenera kulandira katemerayu kupanda kutero, sazaloledwa kugwira ntchito
Posachedwapa, bungwe la zisankho la Meki komanso kampani ya lamya za m’manja ya Tieniemu ndi kampani zina, zauzanso ogwira ntchito ake kuti akuyenera kulandira katemerayu kupanda kutero, sazaloledwa kugwira ntchito
Female
Bungwe la CDEDI Pothilirapo ndemanga kudzera mkalata yomwe yatulutsa masiku ochepa apitawo lati ndi lodabwa ndi kukhala chete kwa boma pa mchitidwewu
Bungwe la sidedi Pothilirapo ndemanga kudzera mkalata yomwe yatulutsa masiku ochepa apitawo lati ndi lodabwa ndi kukhala chete kwa boma pa mchitidwewu
Female
Bambo azaka 29 zakubadwa m’boma la Chiradzulu ali mchitokosi cha apolisi ati kaamba komuganizira kuti wagwililira agogo a zaka 85 zakubadwa omwenso akudwala
Bambo azaka twente naini zakubadwa m’boma la Chiradzulu ali mchitokosi cha apolisi ati kaamba komuganizira kuti wagwililira agogo a zaka eite faifi zakubadwa omwenso akudwala
Female
Malingana ndi malipoti, izi zachitika pa mudzi wa Ntope, mfumu yaikulu Mkalo m’bomalo. Mneneri wa polisi ku Chiradzulu, Innocent Moses
Malingana ndi malipoti, izi zachitika pa mudzi wa Ntope, mfumu yaikulu Mkalo m’bomalo. Mneneri wa polisi ku Chiradzulu, Inosenti Mozesi
Female
wati oganizilidwayu ndi Andrew Mitawa yemwe anapezeleredwa akupalamula mlanduwu ndi mwana wa gogoyu
wati oganizilidwayu ndi Andulu Mitawa yemwe anapezeleredwa akupalamula mlanduwu ndi mwana wa gogoyu
Female
Moses wati mwanayu anakuwa kufunafuna thandizo pomwe anaona zachilendozi ndipo anthu anabwera omwe anagwira Mitawa ndi kukamupereka ku polisi
Mozesi wati mwanayu anakuwa kufunafuna thandizo pomwe anaona zachilendozi ndipo anthu anabwera omwe anagwira Mitawa ndi kukamupereka ku polisi
Female
Kufikira ana komanso achinyamata ndi mauthenga a chilimbikitso komanso okhuza tsogolo lawo labwino, akuti ndi imodzi mwa njira yomwe ingathandize
Kufikira ana komanso achinyamata ndi mauthenga a chilimbikitso komanso okhuza tsogolo lawo labwino, akuti ndi imodzi mwa njira yomwe ingathandize
Female
kuti ana ndi achinyamata azipewa kuchita makhalidwe oipa omwe amasokoneza tsogolo lawo. Izitu ndi malingana ndi gulu la achinyamata la Youth Mindset Change (YMC)
kuti ana ndi achinyamata azipewa kuchita makhalidwe oipa omwe amasokoneza tsogolo lawo. Izitu ndi malingana ndi gulu la achinyamata la yufi maindiseti chenji (wayiemusi)
Female
lomwe kumathero a Sabatayi linakapereka uphungu komanso kukachita ntchito za Chifundo pa malo osamalira ana asowa chisamaliro cha makolo a Chikondi ndi Mphatso Orphanage mu mzinda wa Lilongwe
lomwe kumathero a Sabatayi linakapereka uphungu komanso kukachita ntchito za Chifundo pa malo osamalira ana asowa chisamaliro cha makolo a Chikondi ndi Mphatso ofaneji mu mzinda wa Lilongwe
Female
Poyankhula ndi Ndirande FM pambuyo pa ntchitoyi, mkulu oyendetsa ntchito za gululi mu mzinda wa Lilongwe, Madalitso Chakwela
Poyankhula ndi Ndirande efuemu pambuyo pa ntchitoyi, mkulu oyendetsa ntchito za gululi mu mzinda wa Lilongwe, Madalitso Chakwela
Female
anati bungwe lawo limakhulupilira kuti kugawana mnzeru pakati pa anthu kumathandiza kuti aliyense aziyenda mu njira yoyenerera pa moyo
anati bungwe lawo limakhulupilira kuti kugawana mnzeru pakati pa anthu kumathandiza kuti aliyense aziyenda mu njira yoyenerera pa moyo
Female
Malingana ndi Madalitso, kudzera mu ntchito yomwe gulu lawo likuchita, pali chiyembekezo kuti ana komanso achinyamata ambiri akhala ndi mwai okwaniritsa masomphenya awo
Malingana ndi Madalitso, kudzera mu ntchito yomwe gulu lawo likuchita, pali chiyembekezo kuti ana komanso achinyamata ambiri akhala ndi mwai okwaniritsa masomphenya awo
Female
ngakhale akukumana ndi zokhoma zosiyanasiyana. Mwa zina, gululi linalimbikitsa anawa pa zakufunika kwa maphunziro, ubwino osankha anthu ocheza nawo komanso kukondana pakati pawo
ngakhale akukumana ndi zokhoma zosiyanasiyana. Mwa zina, gululi linalimbikitsa anawa pa zakufunika kwa maphunziro, ubwino osankha anthu ocheza nawo komanso kukondana pakati pawo
Female
Gulu la YMC lomwe linayambira pa tsamba la mchezo la WhatsApp, akuti pakadali pano liri ndi malingaliro ofika patali ndi ntchito zake
Gulu la wayiemusi lomwe linayambira pa tsamba la mchezo la Watsapu, akuti pakadali pano liri ndi malingaliro ofika patali ndi ntchito zake
Female
Gululi pakadali pano liri ndi nthambi zake pafupifupi mzigawo zonse za dziko lino komwe achinyamata amakumana komanso kukambirana zinthu zosiyanasiyana zokhuza moyo wawo
Gululi pakadali pano liri ndi nthambi zake pafupifupi mzigawo zonse za dziko lino komwe achinyamata amakumana komanso kukambirana zinthu zosiyanasiyana zokhuza moyo wawo
Female
Bambo Wa Akazi Atatu Akakhala ku Ndende Kaamba Kogwililira. Mkulu wina m'boma la Thyolo yemwe ali ndi akazi atatu, Bosco Mafupa wa zaka 44
Bambo Wa Akazi Atatu Akakhala ku Ndende Kaamba Kogwililira. Mkulu wina m'boma la Thyolo yemwe ali ndi akazi atatu, Bosiko Mafupa wa zaka fotefolo
Female
amugamula kukhala ku ndende kwa zaka khumi ndi zinai (14), bwalo la milandu litamupeza olakwa pa mlandu ogwililira kangapo konse mwana wake omupeza wa zaka 18
amugamula kukhala ku ndende kwa zaka khumi ndi zinai (fotini), bwalo la milandu litamupeza olakwa pa mlandu ogwililira kangapo konse mwana wake omupeza wa zaka eitini
Female
Nkhaniyi ikuti Mafupa wakhala akugwililira mwanayu kuyambira m’chaka cha 2017 koma mwana-yu akadandaula kwa mai ake, amamulimbikitsa kuti asauze wina aliyense za nkhaniyi ndi chiyembekezo kuti banjali lilemera
Nkhaniyi ikuti Mafupa wakhala akugwililira mwanayu kuyambira m’chaka cha twente seventini koma mwanayu akadandaula kwa mai ake, amamulimbikitsa kuti asauze wina aliyense za nkhaniyi ndi chiyembekezo kuti banjali lilemera
Female
Izitu ndi malingana ndi yemwe amaimira mbali ya boma pa mlanduwu, Ishmael Abubast yemwe anati mwa chitsanzo mchaka cha 2017
Izitu ndi malingana ndi yemwe amaimira mbali ya boma pa mlanduwu, Ishumaeli Abubasiti yemwe anati mwa chitsanzo mchaka cha twente seventini
Female
mkuluyu anagwililira mwanayu pomwe mai ake anapita ku mwambo wa chinamwali ndipo anamuopseza kuti asauze wina aliyense
mkuluyu anagwililira mwanayu pomwe mai ake anapita ku mwambo wa chinamwali ndipo anamuopseza kuti asauze wina aliyense
Female
Abubast anaonjezera kuti mchitidwewu unapitilira mchaka cha 2018 ndipo olakwilidwayu atatopa ndi izi, anadziwitsa achibale ena omwe anachita machawi kukatula nkhaniyi kwa adindo oyenerera
Abubasiti anaonjezera kuti mchitidwewu unapitilira mchaka cha twente eitini ndipo olakwilidwayu atatopa ndi izi, anadziwitsa achibale ena omwe anachita machawi kukatula nkhaniyi kwa adindo oyenerera
Female
Apa ndi pomwe apolisi anamanga Mafupa koma poonekera m’bwalo la milandu anaukana mlanduwu zomwe zinachititsa mbali ya boma kubweretsa mboni zitatu
Apa ndi pomwe apolisi anamanga Mafupa koma poonekera m’bwalo la milandu anaukana mlanduwu zomwe zinachititsa mbali ya boma kubweretsa mboni zitatu
Female
zomwe zinatsimikizira za mchitidwewu ndipo atapezeka olakwa, mkuluyu anati bwalo limupatse chilango chochepa chifukwa ali ndi akazi atatu omwe amadalira iye kumbali ya chithandizo
zomwe zinatsimikizira za mchitidwewu ndipo atapezeka olakwa, mkuluyu anati bwalo limupatse chilango chochepa chifukwa ali ndi akazi atatu omwe amadalira iye kumbali ya chithandizo
Female
Koma Oweruza Patrick Namwale anagamula mkuluyu kukhala ku ndende kwa zaka 14 uku akugwira ntchito ya kalavula gaga
Koma Oweruza Patiliki Namwale anagamula mkuluyu kukhala ku ndende kwa zaka fotini uku akugwira ntchito ya kalavula gaga
Female
Bosco Mafupa ndi wa m’mudzi mwa Chipoloma mfumu yaikulu Changata m’boma lomwelo la Thyolo. Nduna ya kale ya ulimi wa nthilira komanso chitukuko cha mmudzi
Bosiko Mafupa ndi wa m’mudzi mwa Chipoloma mfumu yaikulu Changata m’boma lomwelo la Thyolo. Nduna ya kale ya ulimi wa nthilira komanso chitukuko cha mmudzi
Female
a Charles komanso a Henrie Njoloma ndi a Moses Mwenye omwe bungwe la ACB lawamanga powaganizira kuti akukhuzidwa ndi mchitidwe wa katangale, tsopano atulutsidwa pa bail ya bwalo la milandu
a tchalosi komanso a Henele Njoloma ndi a Mozesi Mwenye omwe bungwe la esibi lawamanga powaganizira kuti akukhuzidwa ndi mchitidwe wa katangale, tsopano atulutsidwa pa belo ya bwalo la milandu
Female
ACB ikuganizira kuti atatuwa , ACB ikuganizira kuti atatuwa kuti anasakaza, kuba komanso kuzembaitsa ndalama za boma zokwana K539,000
esibi ikuganizira kuti atatuwa , esibi ikuganizira kuti atatuwa kuti anasakaza, kuba komanso kuzembaitsa ndalama za boma zokwana faifi handled andi fete naini sauzande kwacha
Female
pozigwiritsa ntchito kulipira zakumwa komanso malo ogona ku lodge ya Ryalls Hotel mu mzinda wa Blantyre
pozigwiritsa ntchito kulipira zakumwa komanso malo ogona ku loji ya layozi hotelo mu mzinda wa Bulantaya
Female
Malingana bungwe la ACB, pali kuganizira kuti ndalama-zi zinagwiritsidwa ntchito pa tsiku lomwe a Mchacha anali ku honeymoon ndi mkazi wawo yemwe anali atangomukwatira kumene
Malingana bungwe la esibi, pali kuganizira kuti ndalamazi zinagwiritsidwa ntchito pa tsiku lomwe a Mchacha anali ku hanemuni ndi mkazi wawo yemwe anali atangomukwatira kumene
Female
ndipo zinaperekedwa ndi bungwe la Lilongwe Water Board komanso unduna wa chitukuko cha madziwu
ndipo zinaperekedwa ndi bungwe la Lilongwe wota bodi komanso unduna wa chitukuko cha madziwu
Female
Oweruza Patrick Chirwa wapereka bail kwa anthuwa pambuyo pa ndalama zokwana K500,000 zomwe aliyense wapereka ngati chikole
Oweruza Patiliki Chirwa wapereka belo kwa anthuwa pambuyo pa ndalama zokwana faifi handiledi sauzande kwacha zomwe aliyense wapereka ngati chikole
Female
Pakadali pano, anthuwa akana milandu yomwe ACB yawatsegulira mogwirizana ndi nkhani-yi. Mneneri wa polisi ya Ntcheu, Hastings Chigalu watsimikiza za ngozi yomwe yachitika pa Tsangano m'bomali
Pakadali pano, anthuwa akana milandu yomwe esibi yawatsegulira mogwirizana ndi nkhaniyi. Mneneri wa polisi ya Ntcheu, Hesiting’izi Chigalu watsimikiza za ngozi yomwe yachitika pa Tsangano m'bomali
Female
Ngakhale zambiri zokhuza ngoziyi siznadziwikebe kufikira pano, a Chigalu ati ngoziyi yachitika m'bandakucha wa lero pomwe galimoto ya mtundu wa truck
Ngakhale zambiri zokhuza ngoziyi siznadziwikebe kufikira pano, a Chigalu ati ngoziyi yachitika m'bandakucha wa lero pomwe galimoto ya mtundu wa thilaki
Female
yaombana ndi galimoto ina yonyamula anthu ndipo pali nkhawa kuti ena mwa anthu omwe akhuzidwa ndi ngoziyi amwalira
yaombana ndi galimoto ina yonyamula anthu ndipo pali nkhawa kuti ena mwa anthu omwe akhuzidwa ndi ngoziyi amwalira
Female
Pali chiwopyezo kuti anthu okwana 1.5 Million avutika ndi njara m’dziko muno izi malingana ndi lipoti lomwe Komiti yowona za momwe chakudya chilili m’dziko muno
Pali chiwopyezo kuti anthu okwana wani pointi faifi miliyoni avutika ndi njara m’dziko muno izi malingana ndi lipoti lomwe Komiti yowona za momwe chakudya chilili m’dziko muno
Female
la Malawi Vulnerability Assessment Committee latulutsa. Lipoti-li likutsutsana ndi zomwe President Lazarus Chakwera komanso Nduna ya za ulimi a Lobin Lowe akakhala akuuza a Malawi
la Malawi vunyulabilite asesimenti komitii latulutsa. Lipoti-li likutsutsana ndi zomwe Pulezidenti Lazalasi Chakwera komanso Nduna ya za ulimi a Lobini Lowe akakhala akuuza a Malawi
Female
kuti m’dziko muno muli chakudya chokwanira komanso palibe munthu yemwe afe ndi njala. Malingana ndi lipotili lomwe wasayinira ndi Mlembi ku Unduna owona za ma pulani a chitukuko, a Winford Masanjala
kuti m’dziko muno muli chakudya chokwanira komanso palibe munthu yemwe afe ndi njala. Malingana ndi lipotili lomwe wasayinira ndi Mlembi ku Unduna owona za ma pulani a chitukuko, a Winifodi Masanjala
Female
mwa anthu omwe akhuzidwe ndi njalawa 1.2 Million mwa iwo ndi wochokera m’madera a midzi. Pali nkhawa yoti anthu angapo amwalira pa ngozi yomwe yachitika pa Tsangano m'boma la Ntcheu
mwa anthu omwe akhuzidwe ndi njalawa wani pointi thu miliyoni mwa iwo ndi wochokera m’madera a midzi. Pali nkhawa yoti anthu angapo amwalira pa ngozi yomwe yachitika pa Tsangano m'boma la Ntcheu
Female
Ngoziyi yakhuza galimoto ya mtundu wa truck ndipo yaombana ndi galimoto ina yonyamula anthu. Malipoti akuti pakadali Pani apolisi ndi achipatala sanafike pa Malo a ngoziwa
Ngoziyi yakhuza galimoto ya mtundu wa thilaki ndipo yaombana ndi galimoto ina yonyamula anthu. Malipoti akuti pakadali Pani apolisi ndi achipatala sanafike pa Malo a ngoziwa
Female
Bwalo la milandu ku Balaka lagamula Erick Chimpeni wa zaka 33 kukakhala ku ndende kwa zaka khumi ndi zinai (14) litamupeza olakwa pa mlandu ogwililira mwana wa zaka 13 zakubadwa
Bwalo la milandu ku Balaka lagamula Eliki Chimpeni wa zaka fetefilii kukakhala ku ndende kwa zaka khumi ndi zinai (fotini) litamupeza olakwa pa mlandu ogwililira mwana wa zaka fetini zakubadwa
Female
Malingana ndi oimira boma pa mlanduwu, Liston Sabola, Chimpeni anapalamula mlanduwu pa 6 August chaka chomwe chino pa nthawi yomwe mwanayi anali yekha pa khomo ndipo anali akuphika chakudya cha madzulo
Malingana ndi oimira boma pa mlanduwu, Lisitoni Sabola, Chimpeni anapalamula mlanduwu pa sikisi ogasiti chaka chomwe chino pa nthawi yomwe mwanayi anali yekha pa khomo ndipo anali akuphika chakudya cha madzulo
Female
Sabola anaonjezera kuti mkuluyu anatengera mwanayu ku bafa komwe anakamugwilira koma Tsoka ilo, munthu wina anawaona yemwe
Sabola anaonjezera kuti mkuluyu anatengera mwanayu ku bafa komwe anakamugwilira koma Tsoka ilo, munthu wina anawaona yemwe
Female
anakatula nkhaniyi kwa Makolo ake omwe sanachedwe koma kukamuneneza ku polisi. Komatu Poonekera m’bwalo la milandu, Erick Chimpeni anaukana mlanduwu
anakatula nkhaniyi kwa Makolo ake omwe sanachedwe koma kukamuneneza ku polisi. Komatu Poonekera m’bwalo la milandu, Eliki Chimpeni anaukana mlanduwu
Female
zomwe zinachititsa mbali ya boma kubweretsa mboni zomwe zinatsimikizira za nkhaniyi
zomwe zinachititsa mbali ya boma kubweretsa mboni zomwe zinatsimikizira za nkhaniyi
Female
Apa, oweruza Philip Chibwana anagamula mkulu-yu yemwe ndi m’mudzi mwa Kadamu mfumu yaikulu Nkaya ku Balaka komweko, kukakhala ku ndende kwa zaka 14
Apa, oweruza filipi Chibwana anagamula mkuluyu yemwe ndi m’mudzi mwa Kadamu mfumu yaikulu Nkaya ku Balaka komweko, kukakhala ku ndende kwa zaka fotini
Female
Bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu lamanga nduna yakale ya za chitukuko cha madzi komanso ulimi wa nthilira, a Charles Mchacha
Bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu lamanga nduna yakale ya za chitukuko cha madzi komanso ulimi wa nthilira, a tchalosi Mchacha
Female
A Mchacha omwenso ndi gavanala wa chipani chotsutsa boma cha DPP ku chigawo cha kum'mwera awamanga powaganizira kuti anagwiritsa ndalama za boma polipilira malo ogona komanso kugula za kumwa
A Mchacha omwenso ndi gavanala wa chipani chotsutsa boma cha Dipipi ku chigawo cha kum'mwera awamanga powaganizira kuti anagwiritsa ndalama za boma polipilira malo ogona komanso kugula za kumwa
Female
ku malo ena ogona alendo mu mzinda wa Blantyre. Bwalo la milandu la Chilobwe First Grade Magistrate mu mzinda wa Lilongwe lalamula bambo wina wazaka 27 zakubadwa, Yohane Jailosi
ku malo ena ogona alendo mu mzinda wa Bulantaya. Bwalo la milandu la Chilobwe fesiti giledi majesitileti mu mzinda wa Lilongwe lalamula bambo wina wazaka twente seveni zakubadwa, Yohane Jailosi
Female
Kukakhala ku ndende kwa zaka 7 kaamba kopezeka olakwa pa mlandu ovulaza malo obisika a mkazi wake
Kukakhala ku ndende kwa zaka seveni kaamba kopezeka olakwa pa mlandu ovulaza malo obisika a mkazi wake
Female
Yemwe amaimira boma pa mlanduwu, Austin Daudi, anawuza bwalo la Milandu kuti a Yohane Jailosi anapalamula mlanduwu pa 30 July m’mudzi mwa Msukuma mfumu yaikulu Kabudula m’bomali
Yemwe amaimira boma pa mlanduwu, ositini Daudi, anawuza bwalo la Milandu kuti a Yohane Jailosi anapalamula mlanduwu pa fete julayi m’mudzi mwa Msukuma mfumu yaikulu Kabudula m’bomali
Female
Malingana ndi a Daudi, a Jailosi anamenya ndi kuvulaza malo obisika a mkazi wawo atawafunsa za komwe anabisa bulangete lake
Malingana ndi a Daudi, a Jailosi anamenya ndi kuvulaza malo obisika a mkazi wawo atawafunsa za komwe anabisa bulangete lake
Female
A Jailosi ati anabisa bulangete la mkazi wakeyu pomuganizira kuti anali pa ubwenzi wa mseli ndi njonda ina
A Jailosi ati anabisa bulangete la mkazi wakeyu pomuganizira kuti anali pa ubwenzi wa mseli ndi njonda ina
Female
Koma powonekera m'bwalo la Milandu, Bambo Jailosi anakana mlandu omenya ndi kuvulaza mkazi wakeyu zomwe zinachititsa oimira boma kobweretsa mboni zomwe zinatsimikizira za nkhaniyi
Koma powonekera m'bwalo la Milandu, Bambo Jailosi anakana mlandu omenya ndi kuvulaza mkazi wakeyu zomwe zinachititsa oimira boma kobweretsa mboni zomwe zinatsimikizira za nkhaniyi
Female
ndipo bwalo linapeza a Jailosi olakwa. Apa Jailosi anapempha mkazi wakeyu kuti amukhululukire ponena kuti satana ndi yemwe anawapangitsa kuti apalamule
ndipo bwalo linapeza a Jailosi olakwa. Apa Jailosi anapempha mkazi wakeyu kuti amukhululukire ponena kuti satana ndi yemwe anawapangitsa kuti apalamule
Female
Koma popereka chigamulo chake, Oweruza Mervis Phoya Sulumba analamula Yohane Jailosi kukakhala ku ndende kuti anthu ena a mtima ngati wakewu atengerepo phunziro
Koma popereka chigamulo chake, Oweruza Mevisi Phoya Sulumba analamula Yohane Jailosi kukakhala ku ndende kuti anthu ena a mtima ngati wakewu atengerepo phunziro
Female
Bwalo la milandu la Limbe First Grade Magistrate lati lizapereka chigamulo chake lachiwiri sabata ya mawa ngati kuli koyenera kutumiza ku bwalo lalikulu la milandu wa polisi wina, Andrew Chagaga
Bwalo la milandu la Limbe fesiti giledi majesitileti lati lizapereka chigamulo chake lachiwiri sabata ya mawa ngati kuli koyenera kutumiza ku bwalo lalikulu la milandu wa polisi wina, Andulu Chagaga
Female
yemwe bwaloli linamupeza olakwa pa mlandu ogwilira kuti akalandire chilango. Chagaga anapeza olakwa pa mlandu ogwilira kawiri konse mtsikana wa zaka 17
yemwe bwaloli linamupeza olakwa pa mlandu ogwilira kuti akalandire chilango. Chagaga anapeza olakwa pa mlandu ogwilira kawiri konse mtsikana wa zaka seventini
Female
yemwe ndi ophunzira pa sukulu ya Malawi University of Business and Applied Sciences (MUBAS) pa nthawi yomwe anali m'chitokosi cha apolisi
yemwe ndi ophunzira pa sukulu ya Malawi yunivesite ofu bizinezi andi apulayidi sayansezi (MUBASI) pa nthawi yomwe anali m'chitokosi cha apolisi
Female
Chagaga anapalamula mlanduwu usiku wa pakati pa 12 ndi 13 December chaka chatha, pomwe apolisi anamugwira ndi amnzake
Chagaga anapalamula mlanduwu usiku wa pakati pa thwelofu ndi fetini DISEMBA chaka chatha, pomwe apolisi anamugwira ndi amnzake
Female
pa ulendo wawo opita ku mwambo wa mapemphero kwa Bvumbwe. M’modzi mwa ma Lawyer a boma pa mlanduwu, Chikondi Chijozi anawuza bwalo kuti a Chigaga ndi munthu oipa
pa ulendo wawo opita ku mwambo wa mapemphero kwa Bvumbwe. M’modzi mwa ma loya a boma pa mlanduwu, Chikondi Chijozi anawuza bwalo kuti a Chigaga ndi munthu oipa
Female
ndipo anapalamula mlandu waukulu kwambiri chonchi akuyenera kulandira chilango chokhwima
ndipo anapalamula mlandu waukulu kwambiri chonchi akuyenera kulandira chilango chokhwima
Female
Malingana ndi Lawyer yu, bwalo la Magistrate lomwe lamva mlanduwu silingapereke chilango chokwanira ponena kuti malamulo akulola bwaloli kupereka chilango chosaposera zaka 14
Malingana ndi loyayu, bwalo la Majesitileti lomwe lamva mlanduwu silingapereke chilango chokwanira ponena kuti malamulo akulola bwaloli kupereka chilango chosaposera zaka fotini
Female
choncho chilango chikuyenera kuchokera ku High Court. Oweruza Jack N’riva wa ku bwalo lalikulu la milandu dzulo wakana Pempho la a Gerald Kazembe a chipani cha Malawi Congress (MCP)
choncho chilango chikuyenera kuchokera ku hayi khoti. Oweruza Jaki N’riva wa ku bwalo lalikulu la milandu dzulo wakana Pempho la a jelsi Kazembe a chipani cha Malawi kngilesi (emusipi)
Female
loti chisankho cha phungu ku dera la Mangochi Monkey Bay chichitikenso ponena kuti a Ralph Joma a DPP sanasankhidwe ngati phungu moyenerera
loti chisankho cha phungu ku dera la Mangochi Monkibe chichitikenso ponena kuti a Rafu Joma a Dipipi sanasankhidwe ngati phungu moyenerera
Female