audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
wayamika mfumu yamzindawu ponena kuti kuonongeka kwa msewu wa Chipasula kumaika miyoyo ya anthu pachiophyezo | wayamika mfumu yamzindawu ponena kuti kuonongeka kwa msewu wa Chipasula kumaika miyoyo ya anthu pachiophyezo | Female | |
A Richard Banda, omwenso ndi khansala wa ward ya Chipasula atsimikizanso kuti pachisankho cha chaka cha mawa azapikisana nawo ngati phungu wanyumba yamalamulo waderali | A Litchadi Banda, omwenso ndi khansala wa wadi ya Chipasula atsimikizanso kuti pachisankho cha chaka cha mawa azapikisana nawo ngati phungu wanyumba yamalamulo waderali | Female | |
Inu anthu azaka izo! Ana ama 2000 sima level anu, mungothapo ndalama chabe. Inuyo ndinu okwatira ndalamazo kadyeni ndi akazi anu kunyumba | Inu anthu azaka izo! Ana ama twu sauzande sima levo anu, mungothapo ndalama chabe. Inuyo ndinu okwatira ndalamazo kadyeni ndi akazi anu kunyumba | Female | |
Umenewo ndiye uthenga waukulu mu nyimbo yatsopano ya Wikise yomwe akuyitcha kuti, Amolo.Amolo ndichidule cha a Molotoni, bambo wa mvula zakale, obadwa malemu Kamuzu Banda akadalamula | Umenewo ndiye uthenga waukulu mu nyimbo yatsopano ya Wikise yomwe akuyitcha kuti, Amolo.Amolo ndichidule cha a Molotoni, bambo wa mvula zakale, obadwa malemu Kamuzu Banda akadalamula | Female | |
Bamboyi wapeza ndalama za ngongole ya NEEF, koma m'malo mochita chitukuko ndi ndalama ya ngongoleyo, akupezeka kuti akuseweletsa ndalamazo malo azinjoyi ndi ana obadwa Facebook itayamba | Bamboyi wapeza ndalama za ngongole ya Nifi, koma m'malo mochita chitukuko ndi ndalama ya ngongoleyo, akupezeka kuti akuseweletsa ndalamazo malo azinjoyi ndi ana obadwa Fesibuku itayamba | Female | |
Pomwe Maskal amakwangula mayimbidwe ake, anabweletsa maluwa osonyeza chikondi aja timati ma, Rose flower, pachingerezi | Pomwe Masiko amakwangula mayimbidwe ake, anabweletsa maluwa osonyeza chikondi aja timati ma, lozi fulawa , pachingerezi | Female | |
Mosaona nkhope, Maskal wagawa ndithu maluwa ochuluka 20 kudutsa, Maka asungwana ndiwo anagwamchikondi ndi maluwawo | Mosaona nkhope, Masiko wagawa ndithu maluwa ochuluka tuwente kudutsa, Maka asungwana ndiwo anagwamchikondi ndi maluwawo | Female | |
Ena koma anadandaula, Ife kuno, Kuno Mukungogawatu mbali imodzi maluwawo Uku maluwawo akugawidwa, anyamata ena nawo anakweza manja awo kuti alandire nawo | Ena koma anadandaula, Ife kuno, Kuno Mukungogawatu mbali imodzi maluwawo Uku maluwawo akugawidwa, anyamata ena nawo anakweza manja awo kuti alandire nawo | Female | |
Munthu atafuna kufunsa kuti nyimbo yomwe anthu anadukula kwambiri pa nyimbo zomwe anayimba Maskal ndi iti, Yankho lake ndilosavuta, Chikondi sindalama | Munthu atafuna kufunsa kuti nyimbo yomwe anthu anadukula kwambiri pa nyimbo zomwe anayimba Maskal ndi iti, Yankho lake ndilosavuta, Chikondi sindalama | Female | |
ija yomwe anayimba ndi anyamata a Biriwiri. Nyimboyi ndiyachangu, ayi anthu anathamangitsa magazi ndithu | ija yomwe anayimba ndi anyamata a Biriwiri. Nyimboyi ndiyachangu, ayi anthu anathamangitsa magazi ndithu | Female | |
Anyamata ataliatali, anyamata osachedwa kudzuka, usiku kukabwera akuba, Piksy ndi Maskal anayankhula moselewula chotero uku akufuna kuyamba nyimbo yawo ija ya CV | Anyamata ataliatali, anyamata osachedwa kudzuka, usiku kukabwera akuba, Pikise ndi Masiko anayankhula moselewula chotero uku akufuna kuyamba nyimbo yawo ija ya sivi | Female | |
Poyambapo, Maskal anayiyimba yekha nyimboyi koma sanachedwe kuvomereza kuti: Nyimboyi siyokoma opanda Piksy. Ayiyimba nyimboyi anyamata awa mpaka anthu akhutira, nawo asungwana poyipatsa moto avekere Indze | Poyambapo, Masiko anayiyimba yekha nyimboyi koma sanachedwe kuvomereza kuti: Nyimboyi siyokoma opanda Pikise. Ayiyimba nyimboyi anyamata awa mpaka anthu akhutira, nawo asungwana poyipatsa moto avekere Indze | Female | |
Nyimbo ya Maskal ya 2010, Hey, sinali nyimbo yachikondi yamasewera. Mawu oti "hey" amayimbidwa mwanthetemwa | Nyimbo ya Maskal ya twente teni, Heyi, sinali nyimbo yachikondi yamasewera. Mawu oti heyi amayimbidwa mwanthetemwa | Female | |
Uku akuyimba nyimboyi Maskal, akumatha kugwirako mkono wa msungwana uyu apo, komanso uyo apo. Ndiye asungwana ena akuchita kumuyang'ana ndi diso loyitana Kuti gwilaniko mkono wangawu | Uku akuyimba nyimboyi Masiko, akumatha kugwirako mkono wa msungwana uyu apo, komanso uyo apo. Ndiye asungwana ena akuchita kumuyang'ana ndi diso loyitana Kuti gwilaniko mkono wangawu | Female | |
Maskal wayimbapo kale nyimbo zingapo. Mwina ena amakayika kuti munthuyu ku America-ko wakhalitsa, koma Chichewa chituluka chosalala monga chakale muja akadali kuno kudya thendo Komatu ayi ndithu | Masiko wayimbapo kale nyimbo zingapo. Mwina ena amakayika kuti munthuyu ku Amerika-ko wakhalitsa, koma Chichewa chituluka chosalala monga chakale muja akadali kuno kudya thendo Komatu ayi ndithu | Female | |
onerani ka video aka momwe akuyimbira Zili ndi iwe. Paja nyimbo ya Unamata ija ndiyo wamaliza nayo Piksy uja | onerani ka video aka momwe akuyimbira Zili ndi iwe. Paja nyimbo ya Unamata ija ndiyo wamaliza nayo Pikise uja | Female | |
Komabe, asanachokeletu naye anafuna awonetse kuti a band ake nawo ndi aluso. Anyamata azidawa m'modzim'modzi amapatsidwa mpata kuti ayimbe nyimbo yoti anthu agome nayo ndi chida chakecho | Komabe, asanachokeletu naye anafuna awonetse kuti a bandi ake nawo ndi aluso. Anyamata azidawa m'modzim'modzi amapatsidwa mpata kuti ayimbe nyimbo yoti anthu agome nayo ndi chida chakecho | Female | |
Mnyamata oyimba keyboard atapatsidwa mpata, anayimba ija ya Kodi nonse mwasamba, Piksy naye ataona momwe mnyamata wa keyboard-yu wayinyamulira nyimbo imeneyi, anangoyamba kuyilowa | Mnyamata oyimba kibodi atapatsidwa mpata, anayimba ija ya Kodi nonse mwasamba, Piksy naye ataona momwe mnyamata wa keyboard-yu wayinyamulira nyimbo imeneyi, anangoyamba kuyilowa | Female | |
nawo anthu kuyankhira uku akukumbuka zaku sitandade 1 ndi 2 kale lija. Momwe akuyimbira Piksy ndi anyamata a band ake kuno, Ayi ndithu zikusonyeza kuti anthuwa anakonzeka | nawo anthu kuyankhira uku akukumbuka zaku sitandade wani ndi thu kale lija. Momwe akuyimbira Pikise ndi anyamata a bandi ake kuno, Ayi ndithu zikusonyeza kuti anthuwa anakonzeka | Female | |
Nyimbo ija ya Chonchobe mwayikumbukira Anyamata amagitala komanso azawo omwe akuyimba zija zina anachitatu kuyifikitsa pena | Nyimbo ija ya Chonchobe mwayikumbukira Anyamata amagitala komanso azawo omwe akuyimba zija zina anachitatu kuyifikitsa pena | Female | |
Nanga taganizani zida kumadzaziveketsa ngati kuti palowa anyamata ang'oma wagule uja olemekezeka, aja omwe amadziwa kuomba ng'oma yopereka chikoka | Nanga taganizani zida kumadzaziveketsa ngati kuti palowa anyamata ang'oma wagule uja olemekezeka, aja omwe amadziwa kuomba ng'oma yopereka chikoka | Female | |
Ayi ndithu, anthu kuno akusangalala ndi oyimba momwe akuyimbira, komanso nawo azida sakuphweketsa. Atamaliza Onesimus uja, aliyese anali atadziwilatu kuti oyimba otsatira ndi Piksy | Ayi ndithu, anthu kuno akusangalala ndi oyimba momwe akuyimbira, komanso nawo azida sakuphweketsa. Atamaliza Onesimasu uja, aliyese anali atadziwilatu kuti oyimba otsatira ndi Pikise | Female | |
DJ anayimbapo nyimbo zingapo kuti anthu asasungulumwe. Kenaka, oyendetsa mwambowu analengeza kuti Piksy-yo alowe m'bwalo | DiJei anayimbapo nyimbo zingapo kuti anthu asasungulumwe. Kenaka, oyendetsa mwambowu analengeza kuti Pikise-yo alowe m'bwalo | Female | |
Komatu sikuti analowa nthawi yomweyo ayi. A Band yake aliza zida zawo mwina kwa mphindi zoposa zisanu, anthu maso ali cheucheu kudikira kuti amuone | Komatu sikuti analowa nthawi yomweyo ayi. A Bandi yake aliza zida zawo mwina kwa mphindi zoposa zisanu, anthu maso ali cheucheu kudikira kuti amuone | Female | |
Koma sikuti panatha nthawi yayitaliso kwambiri zedi, chimfana chodziwika ndi bomachi chinafika, uku chitayiyambitsa nyimbo yake ija ya Maloto | Koma sikuti panatha nthawi yayitaliso kwambiri zedi, chimfana chodziwika ndi bomachi chinafika, uku chitayiyambitsa nyimbo yake ija ya Maloto | Female | |
Chabopha suti yomwe jekete lake chakongoletsa ndimaphinifolo. Onesimus watsanzika kuti akuyimba nyimbo yake yomaliza, ndipo pa stage pakuyenera kubwera wina | Chabopha suti yomwe jekete lake chakongoletsa ndimaphinifolo. Onesimasi watsanzika kuti akuyimba nyimbo yake yomaliza, ndipo pa siteji pakuyenera kubwera wina | Female | |
Atalengeza choncho, anyamata aband anayambapo zing'wenyeng'wenye za Mr Nobody. Ali mkati mwanyimboyi, Onesimus anafika pena ndikuyamba kufunsa anthu | Atalengeza choncho, anyamata abandi anayambapo zing'wenyeng'wenye za Misita Nobade. Ali mkati mwanyimboyi, Onesimasi anafika pena ndikuyamba kufunsa anthu | Female | |
ngati adavutikapo m'moyo mwawo, ndipo anapempha onse omwe anavutikapo ayatse tochi za mafoni awo, ndipo anthuwa anaveladi | ngati adavutikapo m'moyo mwawo, ndipo anapempha onse omwe anavutikapo ayatse tochi za mafoni awo, ndipo anthuwa anaveladi | Female | |
Pomwe Onesimus amafuna kuyamba kuyimba nyimbo yake ija ya Maria, anapereka funso. Alipo a Maria apa Asungwa ambili anakweza manja kuyankha, Tilipo | Pomwe Onesimus amafuna kuyamba kuyimba nyimbo yake ija ya Mariya, anapereka funso. Alipo a Mariya apa Asungwa ambili anakweza manja kuyankha, Tilipo | Female | |
Koma kuchuluka kwa asungwana omwe anakwezera manjawa mmmh Ndizokayikitsa kuti osewadi akhoza kukhala kuti mayina awo ndi a Maria | Koma kuchuluka kwa asungwana omwe anakwezera manjawa mmmh Ndizokayikitsa kuti osewadi akhoza kukhala kuti mayina awo ndi a Mariya | Female | |
Komatu mwina, asungwanawa amatanthawuza kuti iwowo ndi akhalidwe ngati Maria yemwe Onesimus amamudandaulira munyimboyi | Komatu mwina, asungwanawa amatanthawuza kuti iwowo ndi akhalidwe ngati Mariya yemwe Onesimus amamudandaulira munyimboyi | Female | |
Maria ameneyu amamupempha kuti asafele Benz, asafele fashion ndi zina zoterozo. Uku Onesimus akutsiliza nyimbo yake ija yotamanda namalenga-ija, anthu ena anali akukuwa | Mariya ameneyu amamupempha kuti asafele Benzi, asafele fashoni ndi zina zoterozo. Uku Onesimasi akutsiliza nyimbo yake ija yotamanda namalenga-ija, anthu ena anali akukuwa | Female | |
Panado! Panado!, Ukutu mwina kunali kumupempha kuti awayimbire nyimbo imeneyi, ndipo iyeyu sanazengeleze | Panado! Panado!, Ukutu mwina kunali kumupempha kuti awayimbire nyimbo imeneyi, ndipo iyeyu sanazengeleze | Female | |
Ndiye, uku nyimboyo ili mkati, gulu lomwe lakhala chakutsogolo kwambiri limachita kuyimbilira nawo. Onesimus pamenepo ali mkati moyimba komanso kudzigwedeza | Ndiye, uku nyimboyo ili mkati, gulu lomwe lakhala chakutsogolo kwambiri limachita kuyimbilira nawo. Onesimasi pamenepo ali mkati moyimba komanso kudzigwedeza | Female | |
Anyamata oyesa zida pomwe anadzangoliza zida zawo zonse kuti gwe kupereka uthenga oti nthawi yoyeselera yatha | Anyamata oyesa zida pomwe anadzangoliza zida zawo zonse kuti gwe kupereka uthenga oti nthawi yoyeselera yatha | Female | |
pomweponso oyendetsa mwambowu mpomwe analengeza yakwana nthawi yoti mwambo uyambike. Anthu ambiri anali atalosela kale kuti kukubwera Onesimus | pomweponso oyendetsa mwambowu mpomwe analengeza yakwana nthawi yoti mwambo uyambike. Anthu ambiri anali atalosela kale kuti kukubwera Onesimasi | Female | |
Ndipo mnyamata walusoyo sanataye nthawi, anthu anangova, Ndipita kwawo, kwawo komko Uku akuyenda monyada, kapena tinene kuti monyadilira | Ndipo mnyamata walusoyo sanataye nthawi, anthu anangova, Ndipita kwawo, kwawo komko Uku akuyenda monyada, kapena tinene kuti monyadilira | Female | |
Onesimus, kukuwa kwa asungwana kumachita kumuonjezera moto kuti apitilire kunjanja uku akolowa pa stage-po | Onesimasi, kukuwa kwa asungwana kumachita kumuonjezera moto kuti apitilire kunjanja uku akolowa pa siteji-po | Female | |
Onesimus, Piksy komanso Maskal lero ali ku Illusionz mu mzinda wa Lilongwe, kukumbutsa anthu momwe amkachitira mzaka izo ali ku Nde'feyo entertainment | Onesimasi, Pikise komanso Masiko lero ali ku Ilozhyonzi mu mzinda wa Lilongwe, kukumbutsa anthu momwe amkachitira mzaka izo ali ku Nde'feyo intateinimenti | Female | |
Pomwe pangodutsa mphindi zingapo chikwanileni 10 koloko, ndipomwe gulu lochuluka layamba kufika kuno ku Illuzionz mumzinda wa Lilongwe komwe kuli phwando lamayimbidwe la Nde'feyo Legacy | Pomwe pangodutsa mphindi zingapo chikwanileni teni koloko, ndipomwe gulu lochuluka layamba kufika kuno ku iluzhyonzi mumzinda wa Lilongwe komwe kuli phwando lamayimbidwe la Nde'feyo Legase | Female | |
Nde'feyo mwayikumbuka koma Anyamata aja, omwe adali mu lebo imeneyi, Piksy, Maskal komanso Onesimus nthawi imeneyo akudziwika kuti Armstrong Kalua, lero akumbutsa anthu chikale | Nde'feyo mwayikumbuka koma Anyamata aja, omwe adali mu lebo imeneyi, Pikise, Masiko komanso Onesimasi nthawi imeneyo akudziwika kuti Amusitilong’o Kaluwa, lero akumbutsa anthu chikale | Female | |
Pachipata polowelapa, achitetezo agwidwa nthangwanika ndipo mawu omwe sakuchoka pakamwa pawo ndi a: Cash or ticket | Pachipata polowelapa, achitetezo agwidwa nthangwanika ndipo mawu omwe sakuchoka pakamwa pawo ndi a: kashi or tiketi | Female | |
Ukutu mkufunsa anthu akufikawa ngati alipire ndalama, kapena adadulilatu ticket-yawo. Mkatimo, ife tasuzumiramo ndipo mwakhoma, koma mwambo sunayambe | Ukutu mkufunsa anthu akufikawa ngati alipire ndalama, kapena adadulilatu tiketi-yawo. Mkatimo, ife tasuzumiramo ndipo mwakhoma, koma mwambo sunayambe | Female | |
Zatheka tsopano mwa dongosolo. Katswiri osewera ku tsogolo, Clement Nyondo, wasintha thabwa tsopano pamene walowa timu ya Mighty Wanderers potsatira kuchoka ku timu ya Dedza Dynamos | Zatheka tsopano mwa dongosolo. Katswiri osewera ku tsogolo, kilementi Nyondo, wasintha thabwa tsopano pamene walowa timu ya Maite wandilazi potsatira kuchoka ku timu ya Dedza Dainamozi | Female | |
Nyondo, amene ali ndi zaka 23 ndipo anatenga mphoto ya katakwe omwetsa zigoli zambiri mu TNM Super League ndi zigoli 16 chaka chatha | Nyondo, amene ali ndi zaka twente fili ndipo anatenga mphoto ya katakwe omwetsa zigoli zambiri mu tieni emu supa ligi ndi zigoli sikisitini chaka chatha | Female | |
wasayina mgwirizano wa zaka zitatu ku Lali Lubani kufikira chaka cha 2027. Nkhani ya msamuko wa osewerayu inavuta masiku apitawa | wasayina mgwirizano wa zaka zitatu ku Lali Lubani kufikira chaka cha twente twente seveni. Nkhani ya msamuko wa osewerayu inavuta masiku apitawa | Female | |
pamene bungwe la FAM linanena kuti ali ndi mgwirizano odzatha chaka cha 2025 ku timu ya Dedza Dynamos, koma mwini wake amati mgwirizano wake ukutha pa 5 February chaka chino | pamene bungwe la famu linanena kuti ali ndi mgwirizano odzatha chaka cha twente twente faifi ku timu ya Dedza Dainamozi, koma mwini wake amati mgwirizano wake ukutha pa faifi febuluwale chaka chino | Female | |
Akuluakulu a mbali zonse ziwiri akana kuwulura ndalama zimene asinthana pa malonda a mnyamatayu, koma timu ya Dedza Dynamos inakhazikitsa mtengo wa 15 million Kwacha | Akuluakulu a mbali zonse ziwiri akana kuwulura ndalama zimene asinthana pa malonda a mnyamatayu, koma timu ya Dedza Dainamozi inakhazikitsa mtengo wa fifitini miliyoni kwacha | Female | |
Zinamvekanso kuti Nyondo, amene anadziwika kwambiri ali ku timu ya Karonga United, amafunidwanso ndi ma timu a Singida ya ku Tanzania komanso Kabwe Warriors ya ku Zambia ndinso Silver Strikers | Zinamvekanso kuti Nyondo, amene anadziwika kwambiri ali ku timu ya Karonga yunaitedi, amafunidwanso ndi ma timu a Singida ya ku Tanzaniya komanso Kabwe Waliyazi ya ku Zambiya ndinso siliva sitilaikazi | Female | |
Mtsogoleri wa bungwe la FAM, a Fleetwood Haiya, wapempha oyimbira mpira wa miyendo kuti adzipereke pa ntchito yawo kwinaku akutsatira malamulo a ntchitoyi kuti season ya chaka chino | Mtsogoleri wa bungwe la Famu, a Fulitiwudu Haiya, wapempha oyimbira mpira wa miyendo kuti adzipereke pa ntchito yawo kwinaku akutsatira malamulo a ntchitoyi kuti sizoni ya chaka chino | Female | |
imene iyambe mwezi wa April, ikhale yopambana. A Haiya alankhula izi ku Salima pa mwambo opereka nyota kwa oyimbira 17 | imene iyambe mwezi wa epulo, ikhale yopambana. A Haiya alankhula izi ku Salima pa mwambo opereka nyota kwa oyimbira seventini | Female | |
a mpira wa miyendo komanso ena awiri oyimbira masewero a bitchi soka amene bungwe la FIFA lawayika pa mndandanda wake kuti ayimbira mipikisano ikuluikulu monga COSAFA | a mpira wa miyendo komanso ena awiri oyimbira masewero a bitchi soka amene bungwe la FIFA lawayika pa mndandanda wake kuti ayimbira mipikisano ikuluikulu monga KOSAFA | Female | |
Ena aimbiranso ndime ya chipulula ya World Cup komanso CAF Champions League ndi Confederation Cup. Iwo ati bungwe la FIFA labwenzeretsa ma referee ambiri pa mndandandawu kamba koti likuwakhulupirira | Ena aimbiranso ndime ya chipulula ya Waodi kapu komanso Kafu Tchampiyozi ligi ndi Kofedeleshoni kapu. Iwo ati bungwe la FIFA labwenzeretsa ma rifali ambiri pa mndandandawu kamba koti likuwakhulupirira | Female | |
ndipo iwo abwenze ulemu pogwira ntchitoyi moyikapo mtima komanso kutsatira malamulo amene anaphunzitsidwa kuti adziwagwiritsa ntchito maka akamayimbira mdziko muno | ndipo iwo abwenze ulemu pogwira ntchitoyi moyikapo mtima komanso kutsatira malamulo amene anaphunzitsidwa kuti adziwagwiritsa ntchito maka akamayimbira mdziko muno | Female | |
Ena mwa ma referee amene alandira nyota ndi Easter Zimba, Evans Msonda, Gift Chiko, Godfrey Nkhakananga, Newton Nyirenda, Enes Gumbo | Ena mwa ma rifali amene alandira nyota ndi Esita Zimba, Evansi Msonda, Gifiti Chiko, Godifule Nkhakananga, Nyutoni Nyirenda, Enesi Gumbo | Female | |
Joseph Nyauti, Pondamali Tembo, Clemence Kanduku, Mercy Kayira-Kafoteka, Happiness Mbandambanda, Samuel Fudzulani ndi Lameck Phiri | Jozefe Nyauti, Pondamali Tembo, kilemensi Kanduku, Mese Kayira-Kafoteka, Hapinesi Mbandambanda, Samuele Fudzulani ndi Lameki Phiri | Female | |
Ophunzira wapasukulu ya Exploits University, Khalidah Tuzija wapeleka matumba achimanga okwana 70 andalama zoposa K3 million | Ophunzira wapasukulu ya ekisipuloitsi yunivesite, Khalida Tuzija wapeleka matumba achimanga okwana sevente andalama zoposa fili miliyoni kwacha | Female | |
kwa anthu 700 omwe akhudzika ndi njala m’mudzi wa Manga pansi pamfumu yaikulu Nsamala ku Balaka | kwa anthu seveni handede omwe akhudzika ndi njala m’mudzi wa Manga pansi pamfumu yaikulu Nsamala ku Balaka | Female | |
Ophunzirayu wati akuchita mantha ndi njala yomwe ili m'derali ndipo wakhala akusaka thandizoli kwa anthu akufuna kwabwino kuti afikire anthuwa | Ophunzirayu wati akuchita mantha ndi njala yomwe ili m'derali ndipo wakhala akusaka thandizoli kwa anthu akufuna kwabwino kuti afikire anthuwa | Female | |
Iye wati akufuna anthuwa apeze populumukira, akagawana chimangachi chomwe akuwapatsa cholemera makilogalamu khumi munthu aliyense | Iye wati akufuna anthuwa apeze populumukira, akagawana chimangachi chomwe akuwapatsa cholemera makilogalamu khumi munthu aliyense | Female | |
Mayi Edina Wailesi omwe apindula nawo ndi chimangachi ati akumakhala masiku ena osadya kamba koti alibe chakudya komanso kuti akumadalira maganyu kuti apeze chakudya | Mayi Edina Wailesi omwe apindula nawo ndi chimangachi ati akumakhala masiku ena osadya kamba koti alibe chakudya komanso kuti akumadalira maganyu kuti apeze chakudya | Female | |
Achinyamata 6 mwa 21 omwe analephela kunyamuka nawo lachitatu lapitali kupita m'dziko la Israel kukagwira ntchito za m'minda anyamuka lero pa bwalo la Ndege la Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe | Achinyamata sikisi mwa twente wani omwe analephela kunyamuka nawo lachitatu lapitali kupita m'dziko la izilaeli kukagwira ntchito za m'minda anyamuka lero pa bwalo la Ndege la Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe | Female | |
Mkulu wa kampani ya Workers for Arava Farmers a Justice Kangulu watsimikiza za nkhaniyi polankhula ndi Zodiak powonjezera kuti achinyamatawa adutsira ku Kenya komanso Dubai ndipo akuyembekezeka kufika ku Israel mawa lamulungu | Mkulu wa kampani ya wekazi fo alava famazi a Jusitisi Kangulu watsimikiza za nkhaniyi polankhula ndi Zodiyaki powonjezera kuti achinyamatawa adutsira ku Kenya komanso Dubayi ndipo akuyembekezeka kufika ku Izilaeli mawa lamulungu | Female | |
Iwo awonjezelanso kuti omwe atsala asataye chikhulupiliro kaamba koti akukonzaso dongosolo la ulendo wawo | Iwo awonjezelanso kuti omwe atsala asataye chikhulupiliro kaamba koti akukonzaso dongosolo la ulendo wawo | Female | |
Achinyamata ena 119 ananyamuka lachitatu lapitali pansi pa ndondomeko ya boma yotumiza anthuwa ku Israel kukagwira ntchito za m'minda | Achinyamata ena wani handede andi naintini ananyamuka lachitatu lapitali pansi pa ndondomeko ya boma yotumiza anthuwa ku Izilaeli kukagwira ntchito za m'minda | Female | |
Ophunzira 30 pa sukulu ya sekondare ya Seven Hills pa Chimbiya ku Dedza salemba nawo mayeso a MANEB a Form 2 ndi Form 4 kaamba koti mphunzitsi wa mkulu pasukuluyi anawadyera ndalama zawo za mayeso | Ophunzira fete pa sukulu ya sekondare ya deveni hiuzi pa Chimbiya ku Dedza salemba nawo mayeso a manebu a Fomu thu ndi Fomu folo kaamba koti mphunzitsi wa mkulu pasukuluyi anawadyera ndalama zawo za mayeso | Female | |
Ena mwa ophunzirawa auza Zodiak kuti ndizokhumudwitsa kuti mtsogoleri wa sukulu wawo yemwe wawachita chipongwe | Ena mwa ophunzirawa auza zodiyaki kuti ndizokhumudwitsa kuti mtsogoleri wa sukulu wawo yemwe wawachita chipongwe | Female | |
Mwini wake wa sukukuyi a Hawa Ibrahim watsimikiza za nkhaniyi powonjezera kuti mphunzitsiyu anasakaza ndalama za ophunzira 20 ndipo khumi analephera kulipira ndalama ya mayeso | Mwini wake wa sukukuyi a Hawa Ibulahimu watsimikiza za nkhaniyi powonjezera kuti mphunzitsiyu anasakaza ndalama za ophunzira tuwente ndipo khumi analephera kulipira ndalama ya mayeso | Female | |
Iwo ati nkhaniyi anakayitula ku polisi komanso analembera Kalata bungwe la MANEB ndipo anawauza kuti ndizosatheka kuti ophunzirawa alembe nawo mayeso chaka chino | Iwo ati nkhaniyi anakayitula ku polisi komanso analembera Kalata bungwe la manebu ndipo anawauza kuti ndizosatheka kuti ophunzirawa alembe nawo mayeso chaka chino | Female | |
Nduna ya za chuma, a Simplex Chithyola Banda yalonjeza kuti undunawu uwonjezera thumba la ndalama zopita ku ngongole za ulimi kudzera ku bungwe la NEEF kuti alimi ambiri apindule | Nduna ya za chuma, a Simpulekisi Chithyola Banda yalonjeza kuti undunawu uwonjezera thumba la ndalama zopita ku ngongole za ulimi kudzera ku bungwe la Nifi kuti alimi ambiri apindule | Female | |
A Chithyola ati ndi okhutira ndi momwe bungweli lagawira ngongoleyi nyengo ino komanso kuti anthu akubweza bwino | A Chithyola ati ndi okhutira ndi momwe bungweli lagawira ngongoleyi nyengo ino komanso kuti anthu akubweza bwino | Female | |
Iwo alankhula izi poyamba pa ulendo oyendera alimi omwe anatenga ngongole ya ulimi mdera la ku m'mwera kwa boma la Kasungu | Iwo alankhula izi poyamba pa ulendo oyendera alimi omwe anatenga ngongole ya ulimi mdera la ku m'mwera kwa boma la Kasungu | Female | |
Nduna ya za ulimi a Sam Kawale omwe ali nawo pa ulendowu ati ulimi ndi phata la chuma cha dziko lino kotero kuti kuthandiza alimi ndi mwayi wa ngongole kungachititse kuti dziko lino lithetse njala komanso umphawi mosavuta | Nduna ya za ulimi a Samu Kawale omwe ali nawo pa ulendowu ati ulimi ndi phata la chuma cha dziko lino kotero kuti kuthandiza alimi ndi mwayi wa ngongole kungachititse kuti dziko lino lithetse njala komanso umphawi mosavuta | Female | |
Mkulu wa bungwe la NEEF a Humphrey Mdyetseni wati kudzafika tsiku la lero bungweli lapereka ngongole zokwana K92 billion kwa abizinesi komanso alimi mmadera onse mdziko muno | Mkulu wa bungwe la NEfi a Humfule Mdyetseni wati kudzafika tsiku la lero bungweli lapereka ngongole zokwana Nainte thu biliyoni kwacha kwa abizinesi komanso alimi mmadera onse mdziko muno | Female | |
Kodi mukugwira nao ntchito mdziko la Israel. Dzafikeni kuno kumudzi ngati Merchant nthawi yanu yobwelera ikakwana | Kodi mukugwira nao ntchito mdziko la Izilaeli. Dzafikeni kuno kumudzi ngati Metchanti nthawi yanu yobwelera ikakwana | Female | |
Gulani malo ku Citizen Real Estate Company olipira pang'onopang'ono kwa miyezi 6. Muli ndi mwayi okonzeratu podzafikira kuno kumudzi | Gulani malo ku sitizeni Riu esiteti kampane olipira pang'onopang'ono kwa miyezi sikisi. Muli ndi mwayi okonzeratu podzafikira kuno kumudzi | Female | |
pogula ma plot a 15 by 30 kapena 18 by 30 ku Kanengo, Nathenje kapena ku Nalikule. Malo amenewa alipafupi ndi tala komanso madzi ndi magetsi zinafikako kale | pogula ma puloti a fifitini bayi fete kapena eitini bsi frtr ku Kanengo, Nathenje kapena ku Nalikule. Malo amenewa alipafupi ndi tala komanso madzi ndi magetsi zinafikako kale | Female | |
Gwirani magobo aphindu, gwiritsani ntchito mwayi uwu mwanzeru ndi moyenera. Tumizani achibale odalirika adzayambe process yi m'malo mwanu | Gwirani magobo aphindu, gwiritsani ntchito mwayi uwu mwanzeru ndi moyenera. Tumizani achibale odalirika adzayambe pulosesi yi m'malo mwanu | Female | |
koma mapepala onse ofunikira, zithunzi ndi ma videos zizitumizidwa kudzera ku E-mail yanu kuti mudziwe chimene mukugula | koma mapepala onse ofunikira, zithunzi ndi ma vidiyozi zizitumizidwa kudzera ku imelo yanu kuti mudziwe chimene mukugula | Female | |
Boma lati liri ndi chikonzero chowunikanso malire a Nkhalango ya Thuma ndi Mua Livurezi ku Dedza kutsatira mikangano yomwe yakhala ilipo ndi anthu ozungulira malowa | Boma lati liri ndi chikonzero chowunikanso malire a Nkhalango ya Thuma ndi Mua Livurezi ku Dedza kutsatira mikangano yomwe yakhala ilipo ndi anthu ozungulira malowa | Female | |
Ogwirizira udindo wa mkulu owona za Nkhalango a Carol Chidzungu wauza Zodiak kuti m'chitidwe wa anthu ena kulowerera mu nkhalango zotetezeka ukuchulukira | Ogwirizira udindo wa mkulu owona za Nkhalango a Kalo Chidzungu wauza Zodiyaki kuti m'chitidwe wa anthu ena kulowerera mu nkhalango zotetezeka ukuchulukira | Female | |
ndipo zimaoneka ngati akuwachitira nkhaza akapereka chilango kwa opalamula. A Chidzungu ati ntchito yowunikanso malire | ndipo zimaoneka ngati akuwachitira nkhaza akapereka chilango kwa opalamula. A Chidzungu ati ntchito yowunikanso malire | Female | |
ayigwiria ndi mafumu,akuluakulu owona za nkhalango,akuluakulu owona za malo komanso nthambi zina zokhudzidwa | ayigwiria ndi mafumu,akuluakulu owona za nkhalango,akuluakulu owona za malo komanso nthambi zina zokhudzidwa | Female | |
Apolisi ku Ntchisi apulumutsa bambo wina wazaka 40 ku anthu okwiya omwe amafuna kumupha pomuganizira kuti wadyetsa anthu atatu onse abanja limodzi | Apolisi ku Ntchisi apulumutsa bambo wina wazaka fote ku anthu okwiya omwe amafuna kumupha pomuganizira kuti wadyetsa anthu atatu onse abanja limodzi | Female | |
chakudya cha poizoni omwe pano agonekedwa pa chipatala chachikulu cha m'bomalo. M'neneri pa polisi ya Ntchisi Salomy Zgambo watsimikiza za nkhaniyi | chakudya cha poizoni omwe pano agonekedwa pa chipatala chachikulu cha m'bomalo. M'neneri pa polisi ya Ntchisi Salome Zyambo watsimikiza za nkhaniyi | Female | |
yomwe akuti yachitika dzulo madzulo m'mudzi wa Nthesa. Malinga ndi a Zgambo malipoti akuonetsa kuti mkuluyu yemwe wakhala ali pa mkangano olimbirana malo ndi mayi ake | yomwe akuti yachitika dzulo madzulo m'mudzi wa Nthesa. Malinga ndi a Zyambo malipoti akuonetsa kuti mkuluyu yemwe wakhala ali pa mkangano olimbirana malo ndi mayi ake | Female | |
adagula masikono ndi shuga ndipo anthu atangomaliza kudya anayamba kusanza. Malinga ndi a Zgambo pakadali pano oganizilidwawayu amumanga | adagula masikono ndi shuga ndipo anthu atangomaliza kudya anayamba kusanza. Malinga ndi a Zyambo pakadali pano oganizilidwawayu amumanga | Female | |
Ophunzira wa sitandade 1 wapa pasukulu ya pulayimale ya Mgathira ku Mzuzu Ephron Banda athamangira naye ku chipatala ataponda waya wamagetsi yemwe amalendewera papolo lina la Escom pasukulupo | Ophunzira wa sitandade 1 wapa pasukulu ya pulayimale ya Mgathira ku Mzuzu Efuloni Banda athamangira naye ku chipatala ataponda waya wamagetsi yemwe amalendewera papolo lina la Esikomu pasukulupo | Female | |
Wachiwiri kwa m'neneli wa polisi ya Mzuzu, a Rose Chiphyola wati izi zachitika pomwe mnyamatayu yemwe ndiwa zaka zisanu ndi ziwiri amasewera ndi anzake lero lachinayi | Wachiwiri kwa m'neneli wa polisi ya Mzuzu, a Rozi Chiphyola wati izi zachitika pomwe mnyamatayu yemwe ndiwa zaka zisanu ndi ziwiri amasewera ndi anzake lero lachinayi | Female | |
Iyi ndi ngozi yachiwili yokhudza mwana kuvulala ndi magetsi, ina yonga yomweyi itachitikanso miyezi isanu ndi imodzi yapitayo ku Mzuzu | Iyi ndi ngozi yachiwili yokhudza mwana kuvulala ndi magetsi, ina yonga yomweyi itachitikanso miyezi isanu ndi imodzi yapitayo ku Mzuzu | Female | |
Mwezi wa August mchaka Cha 2023, mnyamata wa zaka 12 anafa ataponda waya wamagetsi pa sukulu ya Ching'ambo komwe anapita kukaona zotsatira zamayeso a sitandade 8 omwe iye analemba | Mwezi wa osasiti mchaka Cha twente twente fili, mnyamata wa zaka twelofu anafa ataponda waya wamagetsi pa sukulu ya Ching'ambo komwe anapita kukaona zotsatira zamayeso a sitandade eiti omwe iye analemba | Female | |
Pakadali pano kampani ya Escom sinalankhulepo pankhaniyi. Madala Lawi, zawo zimakhala zokuyika m'malingaliro | Pakadali pano kampani ya Esikomu sinalankhulepo pankhaniyi. Madala Lawi, zawo zimakhala zokuyika m'malingaliro | Female | |
Mfundo zokhwima, gitala yokodoledwa bwino. Ndiye muli voice amwene, yomachita kuperekera umboni kuti koma luso ku Malawi kwathu kuno tili nalo | Mfundo zokhwima, gitala yokodoledwa bwino. Ndiye muli voisi amwene, yomachita kuperekera umboni kuti koma luso ku Malawi kwathu kuno tili nalo | Female | |
Muonere video ya Lawi yoyamba chaka chino, Solo, yomwe ikutuluka 7 koloko ino Podina linki iyi Zonse takamba m'mwambazi zikuphera mphongo | Muonere vidiyo ya Lawi yoyamba chaka chino, Solo, yomwe ikutuluka seveni koloko ino Podina linki iyi Zonse takamba m'mwambazi zikuphera mphongo | Female | |
Mafumu asanu ndi anayi omwe ali mozungulira nkhalango yosungira nyama ya Kasungu National Park ayikira kumbuyo ntchito yomwe boma linachita | Mafumu asanu ndi anayi omwe ali mozungulira nkhalango yosungira nyama ya Kasungu Neshono paki ayikira kumbuyo ntchito yomwe boma linachita | Female | |
powonjezera chiwerengero cha nyama m'nkhalango ya Kasungu yomwe ati ikupititsa patsogolo ntchito zokopa alendo | powonjezera chiwerengero cha nyama m'nkhalango ya Kasungu yomwe ati ikupititsa patsogolo ntchito zokopa alendo | Female | |
Iwo atsutsa malipoti omwe nyumba ina yofalitsa nkhani ya mdziko la German idasindikiza | Iwo atsutsa malipoti omwe nyumba ina yofalitsa nkhani ya mdziko la Jelemani idasindikiza | Female | |
kuti ntchitoyi sikupindulira anthu okhala mozungulira nkhalangoyi kaamba ka kuchuluka kwa mkangano pakati pa anthu ndi nyama | kuti ntchitoyi sikupindulira anthu okhala mozungulira nkhalangoyi kaamba ka kuchuluka kwa mkangano pakati pa anthu ndi nyama | Female | |
Mafumuwa motsogozedwa ndi mfumu yayikulu Lukwa ati nyumba yofalitsa nkhani ya ku German yomwe idasindikiza nkhaniyi, idaonetsa kukondera | Mafumuwa motsogozedwa ndi mfumu yayikulu Lukwa ati nyumba yofalitsa nkhani ya ku Jelemani yomwe idasindikiza nkhaniyi, idaonetsa kukondera | Female | |
posafuna maganizo awo komanso boma zokhudza mkangano pakati pa anthu ndi nyama | posafuna maganizo awo komanso boma zokhudza mkangano pakati pa anthu ndi nyama | Female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.