audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Anthu okwiya pa msika wa Chimbiya masanawa agwira abambo awiri omwe apezeka ndi ziphanso za unzika 87 zomwe amafuna kugwiritsa ntchito kugulira fetereza wa AIP
Anthu okwiya pa msika wa Chimbiya masanawa agwira abambo awiri omwe apezeka ndi ziphanso za unzika eite seveni zomwe amafuna kugwiritsa ntchito kugulira fetereza wa Eayipi
Female
A Rabson Chinam'balala awuza Zodiak kuti anthuwa akumazungulira malo ogulitsira fetereza kumakhala ngati akufuna athandize anthu a m'midzi koma akupanga zachinyengo
A Rabisoni Chinam'balala awuza Zodiyaki kuti anthuwa akumazungulira malo ogulitsira fetereza kumakhala ngati akufuna athandize anthu a m'midzi koma akupanga zachinyengo
Female
Iwo ati lero anthu okwiya pa Chimbiya anawachalilira ndipo atasecha m'chikwama chawo anapeza ziphansozi. Pakadali pano anthuwa akawasiya ku polisi ya Linthipe m'bomali
Iwo ati lero anthu okwiya pa Chimbiya anawachalilira ndipo atasecha m'chikwama chawo anapeza ziphansozi. Pakadali pano anthuwa akawasiya ku polisi ya Linthipe m'bomali
Female
M'modzi mwa akuluakulu achipani chotsutsa boma cha DPP a Uladi Mussa omwe amadziwikanso bwino kuti Chenji Golo
M'modzi mwa akuluakulu achipani chotsutsa boma cha Dipipi a Uladi Mussa omwe amadziwikanso bwino kuti Chenji Golo
Female
alengeza kuti atuluka mchipanichi ndipo tsopano alowa chipani cha Malawi Congress Party (MCP)
alengeza kuti atuluka mchipanichi ndipo tsopano alowa chipani cha Malawi kongelesi pate (emusipi)
Female
A Malawi ena adandaula ndikukwera mitengo kwazinthu m'dziko lino komwe akuti kwafika povuta komanso kuwalepheletsa kudya molongosoka
A Malawi ena adandaula ndikukwera mitengo kwazinthu m'dziko lino komwe akuti kwafika povuta komanso kuwalepheletsa kudya molongosoka
Female
Anthuwa omwe tacheza nawo lero kumisika ya Area 18, 47 komanso Kawale ndi Mtandire ati zinthu zikukwera mitengo tsiku ndi tsiku
Anthuwa omwe tacheza nawo lero kumisika ya eliya eitini, foteseveni komanso Kawale ndi Mtandire ati zinthu zikukwera mitengo tsiku ndi tsiku
Female
mwachitsanzo Shuga madera ena ndi 2700 kwacha pomwe bigili ya mbatatesi ndi 10 000 kwacha
mwachitsanzo Shuga madera ena ndi thusauzande sevenihandede kwacha pomwe bigili ya mbatatesi ndi teni sauzande kwacha
Female
A Emily Kaminjolo omwe amagulitsa zakudya zosiyanasiyana pa msika wa ku 18, adandaula kuti akapita kowoda akumapeza kuti mtengo wakatundu wakwera
A Emily Kaminjolo omwe amagulitsa zakudya zosiyanasiyana pa msika wa ku eitini, adandaula kuti akapita kowoda akumapeza kuti mtengo wakatundu wakwera
Female
Pomwe a James ochokera kwa Mtsiliza ati zinthu sizilibwino, Ufa komanso ndiwo zakwera mopitilira, koma ndalama yomwe amalandira idakali chimodzimodzi
Pomwe a Jemusi ochokera kwa Mtsiliza ati zinthu sizilibwino, Ufa komanso ndiwo zakwera mopitilira, koma ndalama yomwe amalandira idakali chimodzimodzi
Female
Bungwe la CFTC lati lakhala likuchita kafukufuku wake kuyambira mwezi wa November za kukwera mitengo kwa zinthu, ndipo posachedwapa board ya bungweli
Bungwe la siefutisi lati lakhala likuchita kafukufuku wake kuyambira mwezi wa Novemba za kukwera mitengo kwa zinthu, ndipo posachedwapa bodi ya bungweli
Female
likumana kuunikira zotsatira za kafukufuku-yi ndi zilango zomwe zikuyenera kupita kwa amalonda omwe akukweza zinthu zawo mopsola muyezo
likumana kuunikira zotsatira za kafukufuku-yi ndi zilango zomwe zikuyenera kupita kwa amalonda omwe akukweza zinthu zawo mopsola muyezo
Female
Khothi la First Grade Magistrate ku Mchinji lalamula a Julius Tsamba azaka 20 kukakhala kundende kwa zaka 14 kamba kogwililira msungwana wa zaka 12
Khothi la fesiti giledi msjesitileti ku Mchinji lalamula a Julius Tsamba azaka tuwente kukakhala kundende kwa zaka fotini kamba kogwililira msungwana wa zaka thwelofu
Female
Bwaloli linamva kudzera kwa woyimira boma pa mlanduwu Sub Inspector Yotamu Chaonaine kuti a Tsamba anawamanga mwezi wa Disembala chaka chatha
Bwaloli linamva kudzera kwa woyimira boma pa mlanduwu sabu insipekita Yotamu Chaonaine kuti a Tsamba anawamanga mwezi wa Disembala chaka chatha
Female
M'chigamulo chake, First Grade Magistrate Yohane Nkhata analamula a Tsamba kuti akakhale kundende kwa zaka 14 komwe akagwire ntchito ya kalavula gaga
M'chigamulo chake, fesiti giledi majesitileti Yohane Nkhata analamula a Tsamba kuti akakhale kundende kwa zaka fotoni komwe akagwire ntchito ya kalavula gaga
Female
A Tsamba amachokera m'mudzi wa Gumulira, mdera la mfumu yayikulu Mabvwere m'boma la Mchinji
A Tsamba amachokera m'mudzi wa Gumulira, mdera la mfumu yayikulu Mabvwere m'boma la Mchinji
Female
Mabanja oposera 500 ku mpoto kwa boma la Dedza lero alandira mbewu ya chinangwa kuchokera Kwa phungu wa delari a a Savel Kafwafwa
Mabanja oposera faifi handiledi ku mpoto kwa boma la Dedza lero alandira mbewu ya chinangwa kuchokera Kwa phungu wa delari a a Savel Kafwafwa
Female
A Kafwafwa awuza Zodiak kuti m'delari njala ikumasautsa anthu chaka ndi chaka n'chifukwa agawa mbewu ya chinangwayi yomwe sifuna fetereza komanso imapilira Ku nyengo yovuta
A Kafwafwa awuza Zodiyaki kuti m'delari njala ikumasautsa anthu chaka ndi chaka n'chifukwa agawa mbewu ya chinangwayi yomwe sifuna fetereza komanso imapilira Ku nyengo yovuta
Female
Mfumu yayikulu Tambala yathokoza kamba ka thandizoli ndipo yati iwonetsetsa kuti banja lili lonse m'dera lake lidzale chinangwa pofuna kuthana ndi njala
Mfumu yayikulu Tambala yathokoza kamba ka thandizoli ndipo yati iwonetsetsa kuti banja lili lonse m'dera lake lidzale chinangwa pofuna kuthana ndi njala
Female
Unduna woona za ntchito lero walengeza kusindikizidwa kwa malipiro atsopano ochepetsetsa kwa ogwira ntchito ena, kuphatikizapo madalayivala a galimoto zikuluzikulu
Unduna woona za ntchito lero walengeza kusindikizidwa kwa malipiro atsopano ochepetsetsa kwa ogwira ntchito ena, kuphatikizapo madalayivala a galimoto zikuluzikulu
Female
Malingana ndi kalata yomwe tawona, madalayivala oyendetsa galimoto zonyamula katundu wolemera matani oposa 30 ndipo amapita kunja kwa dziko lino, adzilandira K230,000 pa mwezi
Malingana ndi kalata yomwe tawona, madalayivala oyendetsa galimoto zonyamula katundu wolemera matani oposa fete ndipo amapita kunja kwa dziko lino, adzilandira thu handiledi andi fete sauzande kwacha pa mwezi
Female
onyamula matani oposa 30 koma m'dziko lomwe lino adzilandira K160,000, pomwe onyamula katundu wosaposera matani 30, malipiro awo atsopano ochepetsetsa, ndi K100,000
onyamula matani oposa fete koma m'dziko lomwe lino adzilandira handiledi andi sikisite sauzande kwacha pomwe onyamula katundu wosaposera matani fete, malipiro awo atsopano ochepetsetsa, ndi handiledi sauzande kwacha
Female
Koma m'modzi mwa akuluakulu a bungwe la madalayivalawa la Truck Drivers Union a Francis Mkandawire wati izi ndi zokhumudwitsa
Koma m'modzi mwa akuluakulu a bungwe la madalayivalawa la Thilaki dilaivazi yunyoni a Fulansisi Mkandawire wati izi ndi zokhumudwitsa
Female
potengera kuti pamodzi ndi owalemba ntchito, omwe ndi a Transporters Association of Malawi, anagwirizana kuti malipiro ochepetsetsa akhale K300,000.00, motero akudabwa chifukwa chomwe boma silinachitire izi
potengera kuti pamodzi ndi owalemba ntchito, omwe ndi a thilansipotazi asosiyeshoni ofu Malawi, anagwirizana kuti malipiro ochepetsetsa akhale fili nandiledi sauzande kwacha motero akudabwa chifukwa chomwe boma silinachitire izi
Female
Undunawu walengezanso kuti malipiro ochepetsetsa m'madera a m'tauni ndi m'modzi akhale K90,000
Undunawu walengezanso kuti malipiro ochepetsetsa m'madera a m'tauni ndi m'modzi akhale nainte sauzande kwacha
Female
ndipo mwa onse, otsikitsitsa ndi ogwira ntchito za pakhomo omwe adzilandira K52, 000
ndipo mwa onse, otsikitsitsa ndi ogwira ntchito za pakhomo omwe adzilandira fifite thu sauzande kwacha
Female
Timu ya masewero a darts, ya Malawi Post Corporation Conference Centre ya ku Blantyre, yakhala katswiri wa mpikisano wa chaka cha 2023
Timu ya masewero a Datsi, ya Malawi Positi kopaleshoni konfelensi senta ya ku Bulantaya, yakhala katswiri wa mpikisano wa chaka cha twente twente fili
Female
umene ndime yake yotsiriza yachitika dzulo ndi lero ku Silver Club House Multipurpose Hall ku Lilongwe
umene ndime yake yotsiriza yachitika dzulo ndi lero ku siliva kilabu hausi matipaposi holo ku Lilongwe
Female
Timuyi, imene yalandira mphoto ya 1.2 million Kwacha, yatolera 27 points pa masiku awiriwa
Timuyi, imene yalandira mphoto ya wani pointi thu miliyoni Kwacha, yatolera twente seveni pointsi masiku awiriwa
Female
ndipo mtsogoleri wa osewera, Carnage Mkandawire, wati chinsinsi cha kupambanaku, chinagona pa kudzipereka komanso mgwirizano
ndipo mtsogoleri wa osewera, kanaje Mkandawire, wati chinsinsi cha kupambanaku, chinagona pa kudzipereka komanso mgwirizano
Female
Timu ya Malawi School of Government-MSG yakhala yachiwiri ndi 21 points ndipo yalandira 800,000 Kwacha
Timu ya Malawi sukulu ofu gavamenti Emuesiji yakhala yachiwiri ndi twente wani pointsi ndipo yalandira 8eiti handiledi sauzande kwacha
Female
pamene Cobbe Barracks yakhala yachitatu ndi 16 points ndipo yalandira 600,000 Kwacha
pamene kobe balakisi yakhala yachitatu ndi sikisitini pointsi ndipo yalandira sikisi handiledi sauzande Kwacha
Female
Mtsogoleri wa bungwe la Darts Association of Malawi, Joe Zangazanga, wati mpikisano unali waukulu pakati pa ma timu
Mtsogoleri wa bungwe la Datsi asosiyeshoni ofu Malawi, Joe Zangazanga, wati mpikisano unali waukulu pakati pa ma timu
Female
kamba koti bank ya CDH Investment inawonjezera ndalama kufika pa 5 million Kwacha kuchoka pa 2 million Kwacha
kamba koti banki ya sidietchi invesitimentsi inawonjezera ndalama kufika pa faifi miliyoni million Kwacha kuchoka pa thu miliyoni Kwacha
Female
Mmodzi mwa akuluakulu a bank ya CDH Investment, Jennie Madinga, wati bank yi iperekanso ndalama za mpikisano wa chaka chino umene ukuyembekezeka kuyamba mwezi wa April
Mmodzi mwa akuluakulu a banki ya sidientchi invesitimentsi , Jeni Madinga, wati banki yi iperekanso ndalama za mpikisano wa chaka chino umene ukuyembekezeka kuyamba mwezi wa epulo
Female
Timu ya Kawinga FC yagonjetsa Namitete Zitha 4-1 mmasewero otsiriza amu league ya mchigawo chapakati
Timu ya Kawinga efusi yagonjetsa Namitete Zitha folo wani mmasewero otsiriza amu ligi ya mchigawo chapakati
Female
ya Chipiku kuti ikhale akatswiri a ligiyi masewero omwe anachitikira pa bwalo la Nankhaka mu mzinda wa Lilongwe lero
ya Chipiku kuti ikhale akatswiri a ligiyi masewero omwe anachitikira pa bwalo la Nankhaka mu mzinda wa Lilongwe lero
Female
Rahim Mtondera wagoletsa zigoli ziwiri pamene Imran Awali ndi Lazarus Chirwa anagoletsa chigoli chimodzi aliyense
Rahimu Mtondera wagoletsa zigoli ziwiri pamene Imurani Awali ndi Lazalasi Chirwa anagoletsa chigoli chimodzi aliyense
Female
Kondwani Nyirenda anagoletsa chigoli chodzichotsera manyazi cha Namitete Zitha. Kawinga FC ndi akatswiri a ligiyi ndi ma point 53 pa masewero 22
Kondwani Nyirenda anagoletsa chigoli chodzichotsera manyazi cha Namitete Zitha. Kawinga efusi ndi akatswiri a ligiyi ndi ma point fifitefili pa masewero twente thu
Female
koma nthambi yoyendetsa mpira mchigawochi yati tsogolo lonse la ukatswiriwu lagona mmanja mwa bungwe la FAM
koma nthambi yoyendetsa mpira mchigawochi yati tsogolo lonse la ukatswiriwu lagona mmanja mwa bungwe la FAMU
Female
Wachiwiri kwa wapampando wa CRFA, Goodall Chinjoka, watiuza kuti komitiyi ipereka lipoti lonse la mmene ligi yayendera ku bungwe la FAM
Wachiwiri kwa wapampando wa sialaefue, Gudo Chinjoka, watiuza kuti komitiyi ipereka lipoti lonse la mmene ligi yayendera ku bungwe la FAMU
Female
ndipo ku Chiwembe ko ndi kumene apange chiganizo ngati Kawinga ili katswiri wa ligi kamba koti masewerowa aseweredwa mkati-kati mwa chipwirikiti cha nkhani ya za chinyengo
ndipo ku Chiwembe ko ndi kumene apange chiganizo ngati Kawinga ili katswiri wa ligi kamba koti masewerowa aseweredwa mkati-kati mwa chipwirikiti cha nkhani ya za chinyengo
Female
Wachiwiri oyamba kwa mtsogoleri wa bungwe la FAM, Christopher Madalitso Kuyera, wati komiti ya bungweli, yowona za mipikisano, iwunikira nkhaniyi ikalandira ma lipoti ochokera ku CRFA
Wachiwiri oyamba kwa mtsogoleri wa bungwe la FAMU, Khilisitofa Madalitso Kuyera, wati komiti ya bungweli, yowona za mipikisano, iwunikira nkhaniyi ikalandira ma lipoti ochokera ku sialaefue
Female
Mwana wazaka 7 Yamikani Witness wafa akulandila thandizo lachipatala ku Machinga atadya chakudya chomwe akuchiganizira kuti munali chiphe
Mwana wazaka seveni Yamikani Witinesi wafa akulandila thandizo lachipatala ku Machinga atadya chakudya chomwe akuchiganizira kuti munali chiphe
Female
Mneneri wachipatala cha Machinga a Wongani Nyirenda, wati mwanayu anali limodzi ndi anthu ena awiri abanja limodzi omwe anafika pachipatalapa lachisanu lapitali
Mneneri wachipatala cha Machinga a Wongani Nyirenda, wati mwanayu anali limodzi ndi anthu ena awiri abanja limodzi omwe anafika pachipatalapa lachisanu lapitali
Female
atadya Nsima yomwe anaphikira ufa wa Gaga. Iwo ati mwana wamwalirayi pamodzi ndi wina yemwe akupitilira kulandira thandizo pachipatalachi anawapezanso ndi nthenda ya Malungo
atadya Nsima yomwe anaphikira ufa wa Gaga. Iwo ati mwana wamwalirayi pamodzi ndi wina yemwe akupitilira kulandira thandizo pachipatalachi anawapezanso ndi nthenda ya Malungo
Female
Apolisi sanayankhulepo pankhaniyi. Chipani chotsutsa boma cha DPP chati ulamuliro wa mgwirizano wa Tonse
Apolisi sanayankhulepo pankhaniyi. Chipani chotsutsa boma cha Dipipi chati ulamuliro wa mgwirizano wa Tonse
Female
uyambe kuchotsera masiku ake okhala m’boma kaamba walephera kutumikira a Malawi Gavanala wachipanichi mchigawo chakumvuma Sheikh Imran Ntenje
uyambe kuchotsera masiku ake okhala m’boma kaamba walephera kutumikira a Malawi Gavanala wachipanichi mchigawo chakumvuma shekhi imulani Ntenje
Female
wati umoyo wa nzika ukupitilira kukhala wa umphawi mu zaka zinayi zomwe utsogoleriwu walamulira dziko lino
wati umoyo wa nzika ukupitilira kukhala wa umphawi mu zaka zinayi zomwe utsogoleriwu walamulira dziko lino
Female
Sheikh Ntenje wati katundu ofunikira monga chimanga, sugar komanso feteleza ndi zina, tsiku ndi tsiku zikukwera mtengo pa msika kusonyeza kulephera kwa boma lilipo panoli
Shekhi Ntenje wati katundu ofunikira monga chimanga, shuga komanso feteleza ndi zina, tsiku ndi tsiku zikukwera mtengo pa msika kusonyeza kulephera kwa boma lilipo panoli
Female
Iwo akuyankhula izi pamalo ochitira malonda a Lizulu m’boma la Ntcheu komwe akuluakulu achipanichi mchigawo chakumvumachi ali pa mdipiti
Iwo akuyankhula izi pamalo ochitira malonda a Lizulu m’boma la Ntcheu komwe akuluakulu achipanichi mchigawo chakumvumachi ali pa mdipiti
Female
omemeza anthu zolembetsa mu kaundula wa kalembera wa unzika. Chisankho cha chaka chamawa cha 2025
omemeza anthu zolembetsa mu kaundula wa kalembera wa unzika. Chisankho cha chaka chamawa cha twente twente faifi
Female
bungwe la chisankho la MEC likuyembekezera kudzagwiritsa ntchito chiphanso cha unzika polemba anthu mukaundula wachisankhochi
bungwe la chisankho la Meki likuyembekezera kudzagwiritsa ntchito chiphanso cha unzika polemba anthu mukaundula wachisankhochi
Female
Ku Ndirande komwe otsatira chipani cha DPP anayimitsa a Kondwani Nankhumwa, anthuwa anakakamiza mkuluyi kuti awayankhule
Ku Ndirande komwe otsatira chipani cha Dipipi anayimitsa a Kondwani Nankhumwa, anthuwa anakakamiza mkuluyi kuti awayankhule
Female
Anthuwa anayimba nyimbo zomwe amapereka uthenga ofunsa kuti, tsono ndikuchotsedwa kwa a Nankhumwa iwo alowere kuti
Anthuwa anayimba nyimbo zomwe amapereka uthenga ofunsa kuti, tsono ndikuchotsedwa kwa a Nankhumwa iwo alowere kuti
Female
M'mawu awo a Nankhumwa ati anthuwa adekhe, kaamba koti sabata ino alongosola bwino lomwe za tsogolo lawo pa ndale
M'mawu awo a Nankhumwa ati anthuwa adekhe, kaamba koti sabata ino alongosola bwino lomwe za tsogolo lawo pa ndale
Female
Achinyamata omwe avala makaka a chipani cha DPP m'dera la Ndirande mu mzinda wa Blantyre akhamukira ndi kutchingira galimoto ya a Kondwani Nankhumwa, uku akuyimba nyimbo zowatamanda
Achinyamata omwe avala makaka a chipani cha Dipipi m'dera la Ndirande mu mzinda wa Bulantaya akhamukira ndi kutchingira galimoto ya a Kondwani Nankhumwa, uku akuyimba nyimbo zowatamanda
Female
A Nankhumwa anali mkachisi wa Makata CCAP komwe kunali mwambo okhazikitsa m'busa Maxwell Ngwaya. Posachedwepa, DPP inachotsa a Nankhumwa mchipanichi
A Nankhumwa anali mkachisi wa Makata sisiepi komwe kunali mwambo okhazikitsa m'busa Makisiwelo Ngwaya. Posachedwepa, Dipipi inachotsa a Nankhumwa mchipanichi
Female
Oyimba wa m'dziko laku South Africa Paige anali akuchita zakumwa zochenjeretsa ndi asungwana ena akwathu komkuno, kuno ku Illusionz mu mzinda wa Lilongwe
Oyimba wa m'dziko laku saufi afilika peji anali akuchita zakumwa zochenjeretsa ndi asungwana ena akwathu komkuno, kuno ku ilizyonzi mu mzinda wa Lilongwe
Female
Koma pomwe anadzangova DJ kuti wayika nyimbo yake ya Ganama, anadzambatuka msungwana waku South Africa-yo, mpaka kuyimilira pa mpando omwe anakhala kuvina mokondwelera zedi
Koma pomwe anadzangova Dijeyi kuti wayika nyimbo yake ya Ganama, anadzambatuka msungwana waku saufi afilika-yo, mpaka kuyimilira pa mpando omwe anakhala kuvina mokondwelera zedi
Female
Uku ndekuti asungwana akwathu kuno akukuwilira, komanso kumusekelera anga adachezapo kale. Paige komanso Driemo anayimba lero kuno ku Illusionz maola angapo apitawo
Uku ndekuti asungwana akwathu kuno akukuwilira, komanso kumusekelera anga adachezapo kale. Peji komanso Diliyemo anayimba lero kuno ku ilizyonzi maola angapo apitawo
Female
Paige wayimba ndithu koma wawasiya anthu akukuwa "One more time! One more time! One more time! Iyeyu wamaliza ndi nyimbo yomwenso a Malawi anayichalira kwambiri "Ghanama
Peji wayimba ndithu koma wawasiya anthu akukuwa "wani mo taimu! wani mo taimu! wani mo taimu! Iyeyu wamaliza ndi nyimbo yomwenso a Malawi anayichalira kwambiri "Ganama
Female
Ndiyetu wayiyimba, komanso wayivina mwadziwindi Ghanamayo. Ndiyekuti pamenepo anthu ena akujambula momwe msungwana walusoyo amadzigwedezera
Ndiyetu wayiyimba, komanso wayivina mwadziwindi Ganamayo. Ndiyekuti pamenepo anthu ena akujambula momwe msungwana walusoyo amadzigwedezera
Female
kwinaku ena akuyimba nawo pokhapo pomangoti: "Ghanama! Ghanama! Ghanama. Ngakhale anthu anayesetsa kumupempha msungwana waku South Africa-yo kuti "One more! One more
kwinaku ena akuyimba nawo pokhapo pomangoti: "Ganama! Ganama! Ganama. Ngakhale anthu anayesetsa kumupempha msungwana waku saufi afilika-yo kuti "wani mo! Wani mo
Female
Ayi ndithu sanabwererenso. Paige uja wayimbapo kale nyimbo zingapo, ndipo wati wagoma ndichikondi cha a Malawi
Ayi ndithu sanabwererenso. Peji uja wayimbapo kale nyimbo zingapo, ndipo wati wagoma ndichikondi cha a Malawi
Female
Wati iye wagoma kuti a Malawi ambiri amadziwa nyimbo zake, chifukwa choti ambiriwa akumayimba nawo mchiyankhulo chachi Zulu chomwe amakonda kuyimba nyimbo zake
Wati iye wagoma kuti a Malawi ambiri amadziwa nyimbo zake, chifukwa choti ambiriwa akumayimba nawo mchiyankhulo chachi Zulu chomwe amakonda kuyimba nyimbo zake
Female
Kenaka anapempha kuti akufuna apereke ulemu kwa Zahara, oyimba wa m'dziko lakwawo ku South Africa uja yemwe anatisiya chaka chatha
Kenaka anapempha kuti akufuna apereke ulemu kwa Zahara, oyimba wa m'dziko lakwawo ku saufi afilika uja yemwe anatisiya chaka chatha
Female
Anthu omwe abwera kuno ku Illuzionz mu mzinda wa Lilongwe akuyipatsa moto. Driemo anafuna ayese zida. Wayimba nyimbo zake zingapo zija zomwe anthu amazikonda zija
Anthu omwe abwera kuno ku iluzyonzi mu mzinda wa Lilongwe akuyipatsa moto. Diliyemo anafuna ayese zida. Wayimba nyimbo zake zingapo zija zomwe anthu amazikonda zija
Female
kenako anadzawathokoza anthu kuti wamaliza kuyimba. Anthu achita kukuwa kuti Ayi Ayi. Atawafunsa kuti nanga bwanji? Gulu lakuwa "Trailer! Trailer! Trailer!
kenako anadzawathokoza anthu kuti wamaliza kuyimba. Anthu achita kukuwa kuti Ayi Ayi. Atawafunsa kuti nanga bwanji? Gulu lakuwa "Thilera! Thilera! Thilera!
Female
DJ Nathan Tunes sanachedwe kuyiyambitsa nyimbo imeneyo. Wayiyimba Driemo pamodzi ndi anthu achimwemwewa ndipo ndiyo watseka nayo mayimbidwe ake
Dijeyi Nafani chunzi sanachedwe kuyiyambitsa nyimbo imeneyo. Wayiyimba Diliyemo pamodzi ndi anthu achimwemwewa ndipo ndiyo watseka nayo mayimbidwe ake
Female
Apa ndiyekuti Paige, posachedwapa akhala akulowa m'bwalo kuno ku Illuzionz mu mzinda wa Lilongwe Driemo anadzangoti "Mesa mumati awa ndi azanga! Azanga! Azanga
Apa ndiyekuti Peji, posachedwapa akhala akulowa m'bwalo kuno ku ilizyonzi mu mzinda wa Lilongwe Diliyemo anadzangoti "Mesa mumati awa ndi azanga! Azanga! Azanga
Female
Anthu omwe akhala kutsogolo kwenikweni ndi stage anali atayiwakhira kale. Kuyimba nawotu modzikhuthura anga kuti, nkhani ili mu nyimboyi idawachitikirapo
Anthu omwe akhala kutsogolo kwenikweni ndi siteji anali atayiwakhira kale. Kuyimba nawotu modzikhuthura anga kuti, nkhani ili mu nyimboyi idawachitikirapo
Female
Munyimbo imeneyo Driemo amakamba za mzako omafunanso akazi ako. Mwachinunu komanso mopanda matukutuku katswiri oyimba Driemo wadutsa mchigulu mwa anthu
Munyimbo imeneyo Diliyemo amakamba za mzako omafunanso akazi ako. Mwachinunu komanso mopanda matukutuku katswiri oyimba Diliyemo wadutsa mchigulu mwa anthu
Female
omwe abwera ku Illusionz mu mzinda wa Lilongwe, ndipo posachedwapa ayambapo kuyimba. Anthu ambiri sanamuzindikirenso kuti wadutsayo ndi Driemo
omwe abwera ku Iluzyonzi mu mzinda wa Lilongwe, ndipo posachedwapa ayambapo kuyimba. Anthu ambiri sanamuzindikirenso kuti wadutsayo ndi Diliyemo
Female
ndipo wadutsadi tikunena pano wakakhala kaye kuchipinda chofikira alendo olemekezeka. Iyeyu asinthana stage ndi oyimba waku South Africa Paige
ndipo wadutsadi tikunena pano wakakhala kaye kuchipinda chofikira alendo olemekezeka. Iyeyu asinthana siteji ndi oyimba waku Saufi afilika Peji
Female
M'modzim'modzi, awiriawiri penaso mwakagulu ndithu, anthu akufika kuno ku Illusionz mu mzinda wa Lilongwe komwe msungwana wa m'dziko la South Africa oyimba mwanthetemwa, Paige, asangalatse anthu
M'modzim'modzi, awiriawiri penaso mwakagulu ndithu, anthu akufika kuno ku ilizyonzi mu mzinda wa Lilongwe komwe msungwana wa m'dziko la Saufi afilika oyimba mwanthetemwa, Peji, asangalatse anthu
Female
Ngakhale nthawi ikuthamangira 9 koloko, kuno anthu akamafika akumakonda kunena kuti:Ahh kudakali m'mawa talawilira
Ngakhale nthawi ikuthamangira naini koloko, kuno anthu akamafika akumakonda kunena kuti:Ahh kudakali m'mawa talawilira
Female
Mkati anthu akuchuluka ndithu. Driemo ndiye oyimba wa dziko lino yemwe asinthane stage ndi Paige-yu
Mkati anthu akuchuluka ndithu. Diliyemo ndiye oyimba wa dziko lino yemwe asinthane stage ndi peji-yu
Female
Kupatula izi, kulinso ma DJ ochuluka omwe achalira kuonetsa luso lawo. Pa zipata zolowera anyamata adzitho ma bouncer sanayambe kutangwanika kwenikweni
Kupatula izi, kulinso ma Dijeyi ochuluka omwe achalira kuonetsa luso lawo. Pa zipata zolowera anyamata adzitho ma baunsa sanayambe kutangwanika kwenikweni
Female
Chigamulo cha nkhani ya za chinyengo zimene zinakhuza ma timu ena a Premier Division, mu ligi ya mchigawo cha pakati, ya Chipiku Stores CRFA Lilongwe and Districts Football League, chatuluka
Chigamulo cha nkhani ya za chinyengo zimene zinakhuza ma timu ena a Pulimiya Divizyoni, mu ligi ya mchigawo cha pakati, ya Chipiku Sitozi sialaefue Lilongwe andi disitilikitsi futubo ligi, chatuluka
Female
Mwazina, Ngolowindo FC ayipatsa chilango choti isasewerenso mu ligiyi kapena kupanga chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi 36
Mwazina, Ngolowindo efusi ayipatsa chilango choti isasewerenso mu ligiyi kapena kupanga chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi fetesikisi
Female
Akuluakulu awiri a timu ya Ngolowindo FC Ibrahim Omar ndi Idrisa Adam awalamula kuti asapangenso chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi 60
Akuluakulu awiri a timu ya Ngolowindo efusi ibulahimu oma ndi Idilisa Adamu awalamula kuti asapangenso chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi sikisite
Female
ndipo mwini wake wa timuyi a Joel Chigona, asapange chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi 24. Akuluakulu awiri a timu ya Namitete Zitha FC
ndipo mwini wake wa timuyi a Jowelo Chigona, asapange chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi twente folo. Akuluakulu awiri a timu ya Namitete Zitha efusi
Female
Akuluakulu awiri a timu ya Namitete Zitha FC Ringo Kanshulu, ndi Wellington Nzunga, asapange chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi 60
Akuluakulu awiri a timu ya Namitete Zitha efusi Ringo Kanshulu, ndi Weling’itoni Nzunga, asapange chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi sikisite
Female
Wapampando wa timu ya Kawinga FC, a Joe Mwase ndi mmodzi mwa akuluakulu a timuyi, Khembo Mogadishu Mumba, asapange chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi 48
Wapampando wa timu ya Kawinga efusi, a Jo Mwase ndi mmodzi mwa akuluakulu a timuyi, Khembo Mogadishu Mumba, asapange chilichonse cha mpira wa miyendo kwa miyezi fote eiti
Female
Bungwe lina la zachifundo la Future for All Malawi laphunzitsa amayi komanso anyamata 100 m’boma la Ntcheu luso lopanga zakudya
Bungwe lina la zachifundo la fyucha fo o Malawi laphunzitsa amayi komanso anyamata wani handiledi m’boma la Ntcheu luso lopanga zakudya
Female
ndi zinthu zina zosiyanasiyana ndicholinga choti anthuwa akhale odzidalira pachuma
ndi zinthu zina zosiyanasiyana ndicholinga choti anthuwa akhale odzidalira pachuma
Female
M’modzi wa akuluakulu kubungweli a Chikondi Phiri wauza Zodiak online kuti munthu yemwe ali ndizochita zomubweretsera chuma
M’modzi wa akuluakulu kubungweli a Chikondi Phiri wauza Zodiyaki onilaini kuti munthu yemwe ali ndizochita zomubweretsera chuma
Female
sikukhala kovuta kutumikira zosowa za umoyo wake komanso pakhomo lake. A Thokozire Tchauya a m’mudzi wa Mingola komanso a Dausi Gwetsani a m’mudzi wa Dzoole
sikukhala kovuta kutumikira zosowa za umoyo wake komanso pakhomo lake. A Thokozire Tchauya a m’mudzi wa Mingola komanso a Dausi Gwetsani a m’mudzi wa Dzoole
Female
mdera la INkosi Kwataine m’bomalo ati maphunzirowa abwera mu nthawi yake. Ndithandizo lochokera ku bungwe la Egmont Trust, amayi ndi anyamatawa
mdera la INkosi Kwataine m’bomalo ati maphunzirowa abwera mu nthawi yake. Ndithandizo lochokera ku bungwe la Egimaunti Thilasiti, amayi ndi anyamatawa
Female
aphunzira kupanga sopo, tomato sosi, jamu ndi kubeka masikono mwa zina
aphunzira kupanga sopo, tomato sosi, jamu ndi kubeka masikono mwa zina
Female
Banja la ufumu wa INkosi Symon Likongwe la m’boma la Neno lili kulikulu la INkosi ya Makhosi Gomani yachisanu
Banja la ufumu wa INkosi Saimoni Likongwe la m’boma la Neno lili kulikulu la INkosi ya Makhosi Gomani yachisanu
Female
m’boma la Ntcheu komwe likukaonetsa a Dalitso Likongwe omwe akuyembekezeka kulowa ufumuwu. Izi ndikutsatira imfa ya INkosi Symon Likongwe mchaka cha 2022
m’boma la Ntcheu komwe likukaonetsa a Dalitso Likongwe omwe akuyembekezeka kulowa ufumuwu. Izi ndikutsatira imfa ya INkosi Saimoni Likongwe mchaka cha twente twente thu
Female
Woimira akubanja lachifumuli, a Zakaliya Mbalati wati pachikhalidwe cha ufumu wa Maseko Ngoni, iwo amayenera awonetse mfumuyi kwa mfumu ya mafumu yi
Woimira akubanja lachifumuli, a Zakaliya Mbalati wati pachikhalidwe cha ufumu wa Maseko Ngoni, iwo amayenera awonetse mfumuyi kwa mfumu ya mafumu yi
Female
Iwo ati zateremu, mothandizidwa ndi INkosi ya Makhosi Gomani yachisanu akaperekano dzinali kwa DC waboma la Neno ndikudikila kuvomeleza kwa dzinali ndi Pulezidenti
Iwo ati zateremu, mothandizidwa ndi INkosi ya Makhosi Gomani yachisanu akaperekano dzinali kwa Disi waboma la Neno ndikudikila kuvomeleza kwa dzinali ndi Pulezidenti
Female
Komiti yosungitsa mwambo ya nthambi yoyendetsa mpira mchigawo cha pakati, ya Central Region Football League (CRFA )yati itulutsa chigamulo cha nkhani ya za chinyengo
Komiti yosungitsa mwambo ya nthambi yoyendetsa mpira mchigawo cha pakati, ya sentilo lijoni futubo ligi (sialaefue )yati itulutsa chigamulo cha nkhani ya za chinyengo
Female
chimene chakhuza ma timu ena a Premier Division mu ligi ya Chipiku Stores pasanadutse ma ola 48
chimene chakhuza ma timu ena a pulimiya divizyoni mu ligi ya Chipiku Sitozi pasanadutse ma ola fote eiti
Female
Komitiyi lero, pa maso pa nthumwi za ma timu a Kawinga FC, Ngolowindo, Namitete Zitha komanso akuluakulu a CRFA, yawerenga zotsatira za kafukufuku amene yapeza mu sabata zitatu zapitazo
Komitiyi lero, pa maso pa nthumwi za ma timu a Kawinga efusi, Ngolowindo, Namitete Zitha komanso akuluakulu a sialaefie, yawerenga zotsatira za kafukufuku amene yapeza mu sabata zitatu zapitazo
Female
Munthu wina, Rashid Likumbo, amene anabwereketsa osewera ake ku timu ya Ngolowindo FC, ndi amene anawulura kuti, usiku wa pa 6 Januwale
Munthu wina, Rashidi Likumbo, amene anabwereketsa osewera ake ku timu ya Ngolowindo efusi, ndi amene anawulura kuti, usiku wa pa sikisi Januwale
Female
panachitika zachinyengo pakati pa akuluakulu ena a timu ya Kawinga FC komanso Ngolowindo yaku Salima kuti Ngolowindo isasewere ndi Namitete Zitha ku Lilongwe
panachitika zachinyengo pakati pa akuluakulu ena a timu ya Kawinga efusi komanso Ngolowindo yaku Salima kuti Ngolowindo isasewere ndi Namitete Zitha ku Lilongwe
Female