audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Mfumu Lukwa yati ikukhulupirira kuti amene analemba nkhaniyi akufuna kuti anthu omwe amathandiza dziko lino
Mfumu Lukwa yati ikukhulupirira kuti amene analemba nkhaniyi akufuna kuti anthu omwe amathandiza dziko lino
Female
ade kukhosi ndi cholinga chofuna kusokoneza ntchito yobwerezetsa za chilengedwe nkhalango yosungira nyama ya Kasungu
ade kukhosi ndi cholinga chofuna kusokoneza ntchito yobwerezetsa za chilengedwe nkhalango yosungira nyama ya Kasungu
Female
Mafumuwa anachititsa msonkhano wa atolankhani m'bomali. Unduna wazaulimi wati anthu 92 mwa anthu 100 aliwonse omwe akuyenera kupindula ndi ndondomeko ya boma
Mafumuwa anachititsa msonkhano wa atolankhani m'bomali. Unduna wazaulimi wati anthu nainte thu mwa anthu wani handiledi aliwonse omwe akuyenera kupindula ndi ndondomeko ya boma
Female
yazipangizo zotsika mtengo ya AIP agula kale zipangizozi. Nduna mu undunawu a Sam Kawale ndiyo yanena izi lero
yazipangizo zotsika mtengo ya Eayipi agula kale zipangizozi. Nduna mu undunawu a Samu Kawale ndiyo yanena izi lero
Female
pomwe iwo limodzi ndi nduna yazofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu komanso akuluakulu a bungwe la boma lobwereketsa ndalama la NEEF anakayendera munda wa senior chief Khongoni ku Lilongwe
pomwe iwo limodzi ndi nduna yazofalitsa nkhani a Mozesi Kunkuyu komanso akuluakulu a bungwe la boma lobwereketsa ndalama la Nifi anakayendera munda wa seniyo tchifi Khongoni ku Lilongwe
Female
Komabe a Kawale ati malo ogulitsira zipangizozi akhalabe otsegula kufikira anthu ena otsalawa atagula zipangizo zawo mundondomekoyi
Komabe a Kawale ati malo ogulitsira zipangizozi akhalabe otsegula kufikira anthu ena otsalawa atagula zipangizo zawo mundondomekoyi
Female
A senior chief Khongoni ndi mmodzi mwa anthu omwe apindula ndi ngongole ya bungwe la NEEF chifukwa anabwereka K15 Million yomwe yawathandiza kulimira mbewu monga chimanga, Soya komanso mtedza
A seniyo tchifi Khongoni ndi mmodzi mwa anthu omwe apindula ndi ngongole ya bungwe la Nifi chifukwa anabwereka fifitini miliyoni kwachz yomwe yawathandiza kulimira mbewu monga chimanga, Soya komanso mtedza
Female
Ulendo wa atolankhaniwu awukonza ndicholinga chofuna kuona momwe anthu akupindulira ndi ngongole ya NEEF, pomwe boma likuchepetsa chiwerengero cha anthu opindula ndi AIP
Ulendo wa atolankhaniwu awukonza ndicholinga chofuna kuona momwe anthu akupindulira ndi ngongole ya Nifi, pomwe boma likuchepetsa chiwerengero cha anthu opindula ndi Eayipi
Female
kuti azitha kupeza thandizo pa ntchito zawo zaulimi mundondomeko za AGCOM komanso minda ikuluikulu ya boma
kuti azitha kupeza thandizo pa ntchito zawo zaulimi mundondomeko za Agikomu komanso minda ikuluikulu ya boma
Female
Timu ya Dedza Dynamos yasankha a Andrew Bunya ngati mphunzitsi wa tsopano wa timuyi. M'modzi mwa akuluakulu a timuyi a Massa Kalamula atsimikiza izi polankhula ndi Zodiak
Timu ya Dedza Dainamozi yasankha a Andulu Bunya ngati mphunzitsi wa tsopano wa timuyi. M'modzi mwa akuluakulu a timuyi a Masa Kalamula atsimikiza izi polankhula ndi Zodiyaki
Female
A Bunya alowa m'malo mwa a Gilbert Chirwa kutsatira kutha kwa mgwirizano wawo ndi timuyi. Timu ya Dedza Dynamos inatsiliza panambala 7 ndi mapointi 38 mu league ya TNM chaka chapitachi
A Bunya alowa m'malo mwa a Gilibati Chirwa kutsatira kutha kwa mgwirizano wawo ndi timuyi. Timu ya Dedza Dainamozi inatsiliza panambala seveni ndi mapointi fete eiti mu ligi ya Tieniemu chaka chapitachi
Female
Pothandiza boma kutukula maphunziro mdziko lino, mai wina wachifundo wadzipereka kugwira ntchito ndi bungwe la Malawi National Spelling Bee
Pothandiza boma kutukula maphunziro mdziko lino, mai wina wachifundo wadzipereka kugwira ntchito ndi bungwe la Malawi Neshono sipeling’i Bi
Female
lomwe limapangitsa mpikisano otchula malemba a mau osiyanasiyana ndicholinga cholimbikitsa ana kudziwa kutchula mawu, kulemba, komaso kukonda kuwerenga
lomwe limapangitsa mpikisano otchula malemba a mau osiyanasiyana ndicholinga cholimbikitsa ana kudziwa kutchula mawu, kulemba, komaso kukonda kuwerenga
Female
Mai Linley Saka Master, adzipeleka kugulira unifolomu ana onse opikisana mumpikisanowu m’dziko lino
Mai Linile Saka Masita, adzipeleka kugulira unifolomu ana onse opikisana mumpikisanowu m’dziko lino
Female
Mai Saka aku Lilongwe, anawonetsa chidwichi atawonela pa kanema wa Zodiak ana ochokela ku Dowa akupikisana kudera komwe bungwe la World Vision likugwira ntchito
Mai Saka aku Lilongwe, anawonetsa chidwichi atawonela pa kanema wa Zodiyaki ana ochokela ku Dowa akupikisana kudera komwe bungwe la waodi vizhyoni likugwira ntchito
Female
Mai Saka, ati agwira ntchitoyi ndi bungwe la Malawi National Spelling Bee kwa zaka zikudzazi
Mai Saka, ati agwira ntchitoyi ndi bungwe la Malawi neshono sipeling’I Bi kwa zaka zikudzazi
Female
Mbali ziwirizi zikukhulupilira kuti izi zithandiza kuti ana asamachite manyazi ndi komaso asamajombe ku sukulu kamba kosowa inifolomu
Mbali ziwirizi zikukhulupilira kuti izi zithandiza kuti ana asamachite manyazi ndi komaso asamajombe ku sukulu kamba kosowa inifolomu
Nyumba yowulutsa mau ya Zodiak ili pa ubale ndi bungwe la Malawi National Spelling Bee
Nyumba yowulutsa mau ya Zodiyaki ili pa ubale ndi bungwe la Malawi Neshono sipeling’I Bi
Female
Ofesi yoona za chisamaliro cha anthu ku Kasungu yati mchitidwe okwatiwitsa ana achichepere ukupitilira kuyika pa chiopsezo tsogolo la ana
Ofesi yoona za chisamaliro cha anthu ku Kasungu yati mchitidwe okwatiwitsa ana achichepere ukupitilira kuyika pa chiopsezo tsogolo la ana
Female
pomwe chiwerengero chikuonetsa kuti ana 517 adalowa m'banja chaka chathachi
pomwe chiwerengero chikuonetsa kuti ana faifi handiledi andi seventini adalowa m'banja chaka chathachi
Female
Mkulu wa ofesiyi a Harrison Thindwa wati ngakhale ofesiyi inalimbikitsa ntchito yochotsa anawa ku maukwati ambiri amabwereranso kaamba ka vuto la makolo ena komanso za chuma
Mkulu wa ofesiyi a Halisoni Thindwa wati ngakhale ofesiyi inalimbikitsa ntchito yochotsa anawa ku maukwati ambiri amabwereranso kaamba ka vuto la makolo ena komanso za chuma
Female
Iwo ati mwa ana okwana 441 omwe inawachotsa ku maukwati, ana oposa 120 anabwereranso ku maukwati enanso anabwera ku sukulu
Iwo ati mwa ana okwana folo handiledi andi fote wani omwe inawachotsa ku maukwati, ana oposa handedi andi tuwente anabwereranso ku maukwati enanso anabwera ku sukulu
Female
Wa pampando wa mgwirizano wa mabungwe omwe sia aboma ku Kasungu a Braxton Mazon Banda ati chiwerengerochi chitha kukhala chochepa
Wa pampando wa mgwirizano wa mabungwe omwe sia aboma ku Kasungu a Burakisitoni Mazon Banda ati chiwerengerochi chitha kukhala chochepa
Female
chifukwa vutoli likuoneka kuti lakula kwambiri maaka mmadera akumidzi kaamba koti achinyamata ambiri alibe uthenga oyenera okhudza uchembere ndi ubereki
chifukwa vutoli likuoneka kuti lakula kwambiri maaka mmadera akumidzi kaamba koti achinyamata ambiri alibe uthenga oyenera okhudza uchembere ndi ubereki
Female
Iwo ati mpofunika kugwirana manja pophunzitsa anthu za kuyipa kwa mchitidwe okwatiwitsa ana akanali ang'ono
Iwo ati mpofunika kugwirana manja pophunzitsa anthu za kuyipa kwa mchitidwe okwatiwitsa ana akanali ang'ono
Female
Nthambi yoona za nyengo yati mvula iyambanso kugwa m'dziko muno mawa pa 1 February 2024
Nthambi yoona za nyengo yati mvula iyambanso kugwa m'dziko muno mawa pa wani febuluwale twente twente folo
Female
Mneneri wa nthambiyi a Yobu Kachiwanda wauza Zodiak masana ano kuti mvulayi ikhala ikugwa mwezi onse wa February ndipo n'gamba ikhala patali patali
Mneneri wa nthambiyi a Yobu Kachiwanda wauza Zodiyaki masana ano kuti mvulayi ikhala ikugwa mwezi onse wa Febuluwale ndipo n'gamba ikhala patali patali
Female
Amalawi akhala akuda nkhawa ndi ng'amba yomwe inayamba kuwumitsa mbewu zawo m'minda
Amalawi akhala akuda nkhawa ndi ng'amba yomwe inayamba kuwumitsa mbewu zawo m'minda
Female
Bambo wa zaka 46 a James Charles wafa khoma la dzenje lomwe anakumba ngati mgodi posaka golide m’mbali mwa mtsinje wa Lisungwi litamugwera m’boma la Ntcheu
Bambo wa zaka fotesikisi a Jemusi Tchalosi wafa khoma la dzenje lomwe anakumba ngati mgodi posaka golide m’mbali mwa mtsinje wa Lisungwi litamugwera m’boma la Ntcheu
Female
M’neneri wapolisi m’boma, M’neneri wapolisi m’boma li a Jacob Khembo watsimikiza za nkhaniyi
M’neneri wapolisi m’boma, M’neneri wapolisi m’boma li a Jakobo Khembo watsimikiza za nkhaniyi
Female
A Khembo ati a James omwe anathamangira nawo kuchipatala cha ching’ono cha Phalula kukalandira thandizo la mankhwala koma zavuta kupulumutsa moyo wawo
A Khembo ati a Jamusi omwe anathamangira nawo kuchipatala cha ching’ono cha Phalula kukalandira thandizo la mankhwala koma zavuta kupulumutsa moyo wawo
Female
Malemuwa amachokera m’mudzi wa a Chiwaya mdera la mfumu yayikulu Tsikulamowa m’bomalo
Malemuwa amachokera m’mudzi wa a Chiwaya mdera la mfumu yayikulu Tsikulamowa m’bomalo
Female
A Landlord Gwamba, walengeza za phwando lake la mayimbidwe, The Best of Gwamba Concert, yomwe idzachitike pa 21 September, 2024 ku Civo mu mzinda wa Lilongwe
A Landilodi Gwamba, walengeza za phwando lake la mayimbidwe, ve besiti ofu Gwamba Konseti, yomwe idzachitike pa tuwente wani sepitemba twentetwente folo ku sivo mu mzinda wa Lilongwe
Female
Polengeza kwa atolankhani masanawa a Landlord-wo, ati phwandoli cholinga chake ndikusangalalira zaka 15 zomwe akhala akuyimba
Polengeza kwa atolankhani masanawa a Landilodi-wo, ati phwandoli cholinga chake ndikusangalalira zaka fifitini zomwe akhala akuyimba
Female
Pa phwandolo akuti padzakhala oyimba angapo akunja, koma lero Gwamba walengeza oyimba wa m'dziko la South Africa, kuti ndiye oyimba oyamba wakunja yemwe adzayatse nawo moto pa nthawiyo
Pa phwandolo akuti padzakhala oyimba angapo akunja, koma lero Gwamba walengeza oyimba wa m'dziko la saufi afilika, kuti ndiye oyimba oyamba wakunja yemwe adzayatse nawo moto pa nthawiyo
Female
Kupatula izi, Gwamba walengezanso za nyimbo yomwe akutulutsa mawa 8 koloko mutu wake, Mukadalitsa, Nyimboyi wayiyimba ndi Praise Umali komanso The Kambwiri Sisters
Kupatula izi, Gwamba walengezanso za nyimbo yomwe akutulutsa mawa eiti koloko mutu wake, Mukadalitsa, Nyimboyi wayiyimba ndi Pulezi Umali komanso ve Kambwiri Sisitazi
Female
Msonkhano okambirana kukhazikitsa ndondomeko yolimbana ndi mchitidwe ochitira nkhanza anthu achikulire uli mkati ku Lilongwe
Msonkhano okambirana kukhazikitsa ndondomeko yolimbana ndi mchitidwe ochitira nkhanza anthu achikulire uli mkati ku Lilongwe
Female
Msonkhanowu, umene lakonza ndi bungwe la Malawi Human Rights Commission, wabweretsa pamodzi nthumwi zosiyana-siyana zimene zigawane nzeru zimene zingathandizire kuchepetsa khalidwe lozunza anthu achikulire
Msonkhanowu, umene lakonza ndi bungwe la Malawi hyumani laitsi komishoni, wabweretsa pamodzi nthumwi zosiyana-siyana zimene zigawane nzeru zimene zingathandizire kuchepetsa khalidwe lozunza anthu achikulire
Female
Imfa zambirizi zikukhuzana ndi zikhulupiriro kuti achikulirewa amapanga za ufiti
Imfa zambirizi zikukhuzana ndi zikhulupiriro kuti achikulirewa amapanga za ufiti
Female
Pa zokambiranazi, nthumwi zati chiwopsezo chipitirira kwa anthu amene akuyandikira kukwanitsa zaka 60 ngati sipapezeka njira zothetsera nkhanza, kuzunza komanso kusala okalamba kamba ka zikhulupirirozi
Pa zokambiranazi, nthumwi zati chiwopsezo chipitirira kwa anthu amene akuyandikira kukwanitsa zaka sikisite ngati sipapezeka njira zothetsera nkhanza, kuzunza komanso kusala okalamba kamba ka zikhulupirirozi
Female
Bungwe la Malawi Human Rights Commission lati mchitidwewu ubwenzeretsa mmbuyo mfundo za chitukuko za Sustainable Development Goals za chaka cha 2030 zimene achikulire, amene chiwerengero chawo ndi 4 peresenti ndi mbali yayikulu
Bungwe la Malawi Hyumani laitsi komishoni lati mchitidwewu ubwenzeretsa mmbuyo mfundo za chitukuko za Sustainable Development sasitenabo divelopumenti gozi za chaka cha tuwente fete zimene achikulire, amene chiwerengero chawo ndi folo peresenti ndi mbali yayikulu
Female
Nthumwi za ku msonkhanowu ndi unduna owona kuti palibe kusiyana pa ntchito pakati pa amayi ndi abambo ndi chisamaliro cha anthu, a polisi
Nthumwi za ku msonkhanowu ndi unduna owona kuti palibe kusiyana pa ntchito pakati pa amayi ndi abambo ndi chisamaliro cha anthu, a polisi
Female
atsogoleri a mipingo, akuluakulu a ma bwalo oweruza milandu komanso ma bungwe omwe si a boma
atsogoleri a mipingo, akuluakulu a ma bwalo oweruza milandu komanso ma bungwe omwe si a boma
Female
President Lazarus Chakwera wati ntchito yokozanso mlatho waukulu wa Lilongwe komanso kukuza ina mwa misewu mu mzindawu ibweretsa kusintha pakaonekedwe ka mzindawu
Pulezidenti lazalasi Chakwera wati ntchito yokozanso mlatho waukulu wa Lilongwe komanso kukuza ina mwa misewu mu mzindawu ibweretsa kusintha pakaonekedwe ka mzindawu
Female
A Chakwera alankhula izi mmawawu pomwe amayika mwala wamaziko wa ntchito ya zomangamanga zomwe boma likugwira mwambo omwe unachitikira pamalo pomwe akugwirapo ntchito yomanga mlathowu
A Chakwera alankhula izi mmawawu pomwe amayika mwala wamaziko wa ntchito ya zomangamanga zomwe boma likugwira mwambo omwe unachitikira pamalo pomwe akugwirapo ntchito yomanga mlathowu
Female
Ntchitoyi akuigwira ndi thandizo la ndalama zokwana K37 billion kuchokera ku boma la Japan
Ntchitoyi akuigwira ndi thandizo la ndalama zokwana fete seveni biliyoni kwacha kuchokera ku boma la Japani
Female
Achinyamata 21 sakhala nawo paulendo opita Israel kukagwira ntchito za m'minda kaamba kolephela kufikira zina mwa zowayeneleza pa ulendowu
Achinyamata tuwente wani sakhala nawo paulendo opita Izilaeli kukagwira ntchito za m'minda kaamba kolephela kufikira zina mwa zowayeneleza pa ulendowu
Female
Mkulu wa kampani ya Workers for Arava Farmers a Justice Kangulu wauza Zodiak kuti mwazina iwo alephera pazifukwa zokhudza Visa
Mkulu wa kampani ya wekazi fo alava famazi a Jusitisi Kangulu wauza Zodiyaki kuti mwazina iwo alephera pazifukwa zokhudza Viza
Female
zomwe akuyembekeza kulongosola mwachangu kuti anyamuke pofika loweruka likudzali
zomwe akuyembekeza kulongosola mwachangu kuti anyamuke pofika loweruka likudzali
Female
Malinga ndi a Kangulu achinyamata 119 ndi omwe anyamuke m'bandakucha uno zomwe akuti zikuthandiza kwambiri kuthana ndi vuto lakusowa kwa ntchito komwe kulipo m'dziko muno
Malinga ndi a Kangulu achinyamata handede andi naintini ndi omwe anyamuke m'bandakucha uno zomwe akuti zikuthandiza kwambiri kuthana ndi vuto lakusowa kwa ntchito komwe kulipo m'dziko muno
Female
M'modzi mwa achinyamatawa Terence Kalemba ochokera mu mzinda wa Blantyre komanso Emmanuel Banda waku Area 24 ku Lilongwe
M'modzi mwa achinyamatawa Telensi Kalemba ochokera mu mzinda wa Bulantaya komanso emanuwelo Banda waku eliya tuwente folo ku Lilongwe
Female
omwe akuti ndondomekoyi ikawathandiza kwambiri kupeza luso latsopano komanso kusintha moyo wawo pankhani za chuma
omwe akuti ndondomekoyi ikawathandiza kwambiri kupeza luso latsopano komanso kusintha moyo wawo pankhani za chuma
Female
Achinyamata 119 asonkhana pa bwalo la ndege la Kamuzu ku Lilongwe pomwe akuyembekezeka kunyamuka kupita ku Israel komwe azikagwira ntchito m'minda
Achinyamata handede andi naintini asonkhana pa bwalo la ndege la Kamuzu ku Lilongwe pomwe akuyembekezeka kunyamuka kupita ku Izilaeli komwe azikagwira ntchito m'minda
Female
M'modzi mwa achinyamatawa Terence Kalemba ochokera mu mzinda wa Blantyre wauza Zodiak kuti moyo m'dziko muno wafika powawa ndipo sakanachitira mwina koma kukagwira nawo ntchitozi
M'modzi mwa achinyamatawa Terensi Kalemba ochokera mu mzinda wa Bulantaya wauza Zodiyaki kuti moyo m'dziko muno wafika powawa ndipo sakanachitira mwina koma kukagwira nawo ntchitozi
Female
Emmanuel Banda waku Area 24 ku Lilongwe naye akuti mwayiwu ndiwofunika kwambiri kwa iye kaamba koti wakhala zaka zambiri akusowa ntchito
Emanuwelo Banda waku eliya tuwente folo ku Lilongwe naye akuti mwayiwu ndiwofunika kwambiri kwa iye kaamba koti wakhala zaka zambiri akusowa ntchito
Female
Komiti ya mtsogoleri wa dziko lino yowona za matenda a Covid-19 komanso Cholera yalangiza adindo aza umoyo ku Mchinji kuti asatayilire
Komiti ya mtsogoleri wa dziko lino yowona za matenda a Covidi-naintini komanso kolera yalangiza adindo aza umoyo ku Mchinji kuti asatayilire
Female
ndipo m'malo mwake akhale tcheru popewa kufala kwa matendawa omwe asawutsa kwambiri m'dziko la Zambia
ndipo m'malo mwake akhale tcheru popewa kufala kwa matendawa omwe asawutsa kwambiri m'dziko la Zambiya
Female
Wapampando wa komitiyi Dr. Wilfred Chalamira Nkhoma wati ngakhale kuti boma simunapezeke munthu odwala matenda a cholera
Wapampando wa komitiyi Dokota. Wulufuledi Chalamira Nkhoma wati ngakhale kuti boma simunapezeke munthu odwala matenda a kolera
Female
mkofunikabe kuti adindo akonzekere mokwanira kamba koti aMalawi ochuluka amachezelana ndi nzika za m'dziko la Zambia
mkofunikabe kuti adindo akonzekere mokwanira kamba koti aMalawi ochuluka amachezelana ndi nzika za m'dziko la Zambiya
Female
Iwo alankhula izi lero pomwe ena mwa mamembala akomitiyi anakayendera bomali kuti akawone momwe ntchito yokonzekera kudziteteza kumatenda a cholera ikuyendera
Iwo alankhula izi lero pomwe ena mwa mamembala akomitiyi anakayendera bomali kuti akawone momwe ntchito yokonzekera kudziteteza kumatenda a kolera ikuyendera
Female
Mkulu wa za umoyo ku Mchinji Dr. Yohane Mwale wapempha anthu akufuna kwabwino kuti awathandize ndi zipangizo zokwanira, zomwe zingawathandize kulimbana ndi nthendayi
Mkulu wa za umoyo ku Mchinji Dokota. Yohane Mwale wapempha anthu akufuna kwabwino kuti awathandize ndi zipangizo zokwanira, zomwe zingawathandize kulimbana ndi nthendayi
Female
Mwazina, komitiyi inakayendera chipatala cha Mchinji komanso pachipata cholowera ndikutulukira m'dziko lino
Mwazina, komitiyi inakayendera chipatala cha Mchinji komanso pachipata cholowera ndikutulukira m'dziko lino
Female
Akuluakulu oyang'anila ntchito za Mtukula Pakhomo m'boma la Dedza alengeza kuti tsopano chiwerengero cha anthu omwe adzipindula ndi ndondomekoyi chafika pa 19,000 kuchoka pa 18,000
Akuluakulu oyang'anila ntchito za Mtukula Pakhomo m'boma la Dedza alengeza kuti tsopano chiwerengero cha anthu omwe adzipindula ndi ndondomekoyi chafika pa naintini sauzande kuchoka pa eitini sauzande
Female
Mkulu woyang'anira ntchitoyi m'bomali a Emmanuel Khumba wauza Zodiak kuti ndalama zomwe anthu opindula amalandira nazo zakwera
Mkulu woyang'anira ntchitoyi m'bomali a Emanuwelo Khumba wauza Zodiyaki kuti ndalama zomwe anthu opindula amalandira nazo zakwera
Female
pamene ndalama yoyambira pa mwezi tsopano ndi K8,000 kuchoka pa K4000 ndipo ena omwe amalandira K8,000 tsopano adzilandira K15,000
pamene ndalama yoyambira pa mwezi tsopano ndi Keiti sauzande kwacha kuchoka pafolo sauzande kwacha ndipo ena omwe amalandira eiti sauzande kwacha tsopano adzilandira fifitini sauzande kwacha
Female
Koma iwo adandaula ndi m'chitidwe wa anthu ena omwe akumati akalandira ndalamazi akumamwa mowa mwa uchidakwa komanso ena akumachita zibwenzi
Koma iwo adandaula ndi m'chitidwe wa anthu ena omwe akumati akalandira ndalamazi akumamwa mowa mwa uchidakwa komanso ena akumachita zibwenzi
Female
Ena mwa anthu omwe akupindula ndi ndondomekoyi a Revi Daniel ndi a Binos chitukula ati akwanitsa kugula ziweto
Ena mwa anthu omwe akupindula ndi ndondomekoyi a Revi Daniele ndi a Binosi chitukula ati akwanitsa kugula ziweto
Female
komanso ndalama zomwe akumalandira akumasungitsa ku magulu kuti ichuluke kuti adzichitiranso mabizinesi ena
komanso ndalama zomwe akumalandira akumasungitsa ku magulu kuti ichuluke kuti adzichitiranso mabizinesi ena
Female
M'busa Milwad Nyangulu wa mpingo wa Synagogue Pentecostal lero wapereka matumba 200 achimanga komanso K6 million
M'busa Miliwadi Nyangulu wa mpingo wa Sinagogi Pentekosito lero wapereka matumba thu handede achimanga komanso sikisi miliyoni kwacha
Female
ku malo osungirako ana amasiye a Home of Hope ku Mchinji kuti zithandizire kuthana ndi vuto la njala komanso mavuto azachuma pa malowa
ku malo osungirako ana amasiye a Homu of Hopu ku Mchinji kuti zithandizire kuthana ndi vuto la njala komanso mavuto azachuma pa malowa
Female
Mkulu wa pa malowa m'busa John Chipeta wati thandizoli lafika mu nthawi yake, kaamba koti anatsala ndi matumba anayi okha kuti adyetse ana kwa tsiku limodzi basi
Mkulu wa pa malowa m'busa Joni Chipeta wati thandizoli lafika mu nthawi yake, kaamba koti anatsala ndi matumba anayi okha kuti adyetse ana kwa tsiku limodzi basi
Female
M'modzi mwa akulu akulu ku mpingo wu a Violet Phiri anati mpingo wawo umaphunzitsa za chikondi komanso kupereka, choncho anawona kofunika kuti athandize anawa
M'modzi mwa akulu akulu ku mpingo wu a Vayoleti Phiri anati mpingo wawo umaphunzitsa za chikondi komanso kupereka, choncho anawona kofunika kuti athandize anawa
Female
Chaka chatha, M'busa Nyangulu anaperekanso matumba achimanga komanso ndalama zokwana five million kwacha pa malowa
Chaka chatha, M'busa Nyangulu anaperekanso matumba achimanga komanso ndalama zokwana faivi miliyoni kwacha pa malowa
Female
Malowa anawakhazikitsa m'chaka cha 1998 ndipo amapereka chisamaliro kwa ana amasiye oposa 750
Malowa anawakhazikitsa m'chaka cha naintini nainte eiti ndipo amapereka chisamaliro kwa ana amasiye oposa seveni handede andi fifite
Female
Athu pafupifupi 1000 omwe ali ndi ulumali osaona, ali ndi mwayi oyambiranso kuona kutsatira ntchito yochita opaleshoni ya maso
Athu pafupifupi wani sauzande omwe ali ndi ulumali osaona, ali ndi mwayi oyambiranso kuona kutsatira ntchito yochita opaleshoni ya maso
Female
yomwe madotolo a mdziko la Brazil kudzera ku ofesi ya Kazembe wadzikoli kuno ku Malawi agwile
yomwe madotolo a mdziko la Bulazilu kudzera ku ofesi ya Kazembe wadzikoli kuno ku Malawi agwile
Female
Malinga ndi Dr Breno Travares Nogueira, oimira ofesi yakazembeyi, ntchitoyi ichitika mmyezi iwiri ikudzayi ndipo ndi gawo limodzi la ntchito zingapo mgawo la zaumoyo zomwe dziko la Brazil lithandize
Malinga ndi Dokota Brueno Thilevasi Nuguwela , oimira ofesi yakazembeyi, ntchitoyi ichitika mmyezi iwiri ikudzayi ndipo ndi gawo limodzi la ntchito zingapo mgawo la zaumoyo zomwe dziko la Bulazilu lithandize
Female
Iwo amalankhula izi ku Kamuzu Palace ku Lilongwe lero pomwe amakumana ndi President Lazarus Chakwera komwenso anati dziko la Brazil lithandiza pantchito yokhazikitsa sukulu yaukachenjede yosula madotolo oona zamaso
Iwo amalankhula izi ku Kamuzu Palesi ku Lilongwe lero pomwe amakumana ndi Pulezidentu lazalasi Chakwera komwenso anati dziko la Bulazilu lithandiza pantchito yokhazikitsa sukulu yaukachenjede yosula madotolo oona zamaso
Female
Nduna yazaumoyo mdzikolino a Khumbidze Kandodo Chiponda yati thandizoli ladza munthawi yake pomwe 80 percent ya omwe saona mdzikolino atalandira thandizo lazaumoyo loyenera atha kuyambiranso kuona
Nduna yazaumoyo mdzikolino a Khumbidze Kandodo Chiponda yati thandizoli ladza munthawi yake pomwe eite pelesenti ya omwe saona mdzikolino atalandira thandizo lazaumoyo loyenera atha kuyambiranso kuona
Female
Unduna wa za maphunziro watseka sukulu ya sekondale yogonera konko ya Asungwana ya St Stephanos ku Area 25 mu mzinda wa Lilongwe
Unduna wa za maphunziro watseka sukulu ya sekondale yogonera konko ya Asungwana ya senti sitefanosi ku Eliya tuwente faifi mu mzinda wa Lilongwe
Female
kaamba ka nkhani za umve pa sukuluyi komanso kuti imagwira ntchito popanda chilolezo kuyambira m'chaka cha 2022
kaamba ka nkhani za umve pa sukuluyi komanso kuti imagwira ntchito popanda chilolezo kuyambira m'chaka cha tuwente tuwente thu
Female
Mmodzi mwa akuluakulu ku undunawu Professor Golden Msilimba watiuza kuti pa sukuluyi yomwe anyamata amayendera, zimbudzi ndizosakwanira zomwenso ndizosasamalirika
Mmodzi mwa akuluakulu ku undunawu Pulofesa godeni Msilimba watiuza kuti pa sukuluyi yomwe anyamata amayendera, zimbudzi ndizosakwanira zomwenso ndizosasamalirika
Female
chakudya cha sukuluyi amasungila mu chipinda chomwe atsikana amagonamo komanso chiphaso chake chogwilira ntchito chinatha chaka cha 2021
chakudya cha sukuluyi amasungila mu chipinda chomwe atsikana amagonamo komanso chiphaso chake chogwilira ntchito chinatha chaka cha twente twente wani
Female
Iwo ati zakhala zikuchitika pa sukuluyi ndizoyika moyo wa ophunzira pa chiopsezo maka pa nthawi ino yomwe dziko la Malawi likulimbanabe ndi nthenda ya cholera
Iwo ati zakhala zikuchitika pa sukuluyi ndizoyika moyo wa ophunzira pa chiopsezo maka pa nthawi ino yomwe dziko la Malawi likulimbanabe ndi nthenda ya kolera
Female
Mmodzi mwa akuluakulu pa sukuluyi a Gersom Banda watsimikiza zakutsekedwa kwa sukukuyi ndipo wati akonza zomwe awuzidwa ndi undunawu mu sabata ziwiri zikudzazi
Mmodzi mwa akuluakulu pa sukuluyi a Gesomu Banda watsimikiza zakutsekedwa kwa sukukuyi ndipo wati akonza zomwe awuzidwa ndi undunawu mu sabata ziwiri zikudzazi
Female
Ofesi yowona zaulimi ku Dedza yati ili ndi chiyembekezo kuti alimi a soya m'bomali apeza phindu lochuluka kaamba kakugwa bwino kwa Mvula komanso nyengo yabwino
Ofesi yowona zaulimi ku Dedza yati ili ndi chiyembekezo kuti alimi a soya m'bomali apeza phindu lochuluka kaamba kakugwa bwino kwa Mvula komanso nyengo yabwino
Female
Wachiwiri kwa mkulu owona za ntchitoyi m'bomali a Ayana Chikankheni watsimikiza za nkhaniyi polankhula ndi Zodiak powonjezera kuti chaka chapitachi zokolora zinachepa kaamba kakusokonekera kwa nyengo
Wachiwiri kwa mkulu owona za ntchitoyi m'bomali a Ayana Chikankheni watsimikiza za nkhaniyi polankhula ndi Zodiyaki powonjezera kuti chaka chapitachi zokolora zinachepa kaamba kakusokonekera kwa nyengo
Female
Koma iwo ati chiwerengero cha alimi a m'ma esiteti omwe alima soya chatsika kuchoka pa mahekitala 251 kufika pa 219
Koma iwo ati chiwerengero cha alimi a m'ma esiteti omwe alima soya chatsika kuchoka pa mahekitala thuhandede andi fifite wani kufika pa thu handede andi naintini
Female
M'modzi mwa alimiwa a Ireen Gama ati iyi ndi nkhani yabwino ngakhale kuti alima soya ekala imodzi yokha chaka chino
M'modzi mwa alimiwa a Ireen Gama ati iyi ndi nkhani yabwino ngakhale kuti alima soya ekala imodzi yokha chaka chino
Female
Achinyamata okwana 140 akuyembekezeka kunyamuka mdziko muno lachitatu kupita ku Israel komwe azikagwira ntchito ku minda
Achinyamata okwana handede andi fote akuyembekezeka kunyamuka mdziko muno lachitatu kupita ku Izilaeli komwe azikagwira ntchito ku minda
Female
A Justice Kangulu omwe ndi mkulu wa kampani yopezera anthu ntchitto ya Arama yomwe ikuyendetsa ntchitoyi, atsimikiza kuti achinyamatawa akuyembekezeka kunyamuka pa bwalo la Kamuzu kupita ku Israel m'bandakucha wa lachitatu
A Jusitisi Kangulu omwe ndi mkulu wa kampani yopezera anthu ntchitto ya Arama yomwe ikuyendetsa ntchitoyi, atsimikiza kuti achinyamatawa akuyembekezeka kunyamuka pa bwalo la Kamuzu kupita ku Izilaeli m'bandakucha wa lachitatu
Female
Iwo ati pomwe amasayina mgwirizano wa ntchito, achinyamatawo awalongosolera mwa mvemvemve, zomwe akuyenera kuyembekezera komanso zomwe mabwana awo akuyembekezera akapita ku Israel
Iwo ati pomwe amasayina mgwirizano wa ntchito, achinyamatawo awalongosolera mwa mvemvemve, zomwe akuyenera kuyembekezera komanso zomwe mabwana awo akuyembekezera akapita ku Izilaeli
Female
Malinga ndi nduna yofalitsa nkhani mdziko muno a Moses Kunkuyu, achinyamata oposa 700 ochokera mdziko muno ali ku Israel komwe akugwira ntchito mu ndondomeko yotumiza ogwira ntchito mmaiko ena
Malinga ndi nduna yofalitsa nkhani mdziko muno a Mozesi Kunkuyu, achinyamata oposa seveni handiledi ochokera mdziko muno ali ku Izilaeli komwe akugwira ntchito mu ndondomeko yotumiza ogwira ntchito mmaiko ena
Female
Wolankhulapo pa nkhani za ufulu, a Michael Kayiyatsa ati pomwe ndondomekoyi ndi yabwino, boma likuyenera kumachita machawi kufotokozera anthu momwe ntchito yotumiza achinyamata ku Israel ikuyendera kuopa manong'onong'o
Wolankhulapo pa nkhani za ufulu, a Maiko Kayiyatsa ati pomwe ndondomekoyi ndi yabwino, boma likuyenera kumachita machawi kufotokozera anthu momwe ntchito yotumiza achinyamata ku Izilaeli ikuyendera kuopa manong'onong'o
Female
bambo wa zaka 46 wafa pa ngozi yapa msewu lero pomwe njinga yake ya moto inawombana ndi galimoto m'mudzi wa Ashani m'boma Mchinji
bambo wa zaka fote sikisi wafa pa ngozi yapa msewu lero pomwe njinga yake ya moto inawombana ndi galimoto m'mudzi wa Ashani m'boma Mchinji
Female
Apolisi ati bamboyu ndi a Gamaliel Keyala am'mudzi wa Mkanda mdera la mfumu yayikulu Mkanda m'bomali
Apolisi ati bamboyu ndi a Gamalielo Keyala am'mudzi wa Mkanda mdera la mfumu yayikulu Mkanda m'bomali
Female
Malemu Keyala amalowera dera la Kapiri kuchoka kwa Kamwendo mu msewu wa Mchinji-Kasungu M18, atakweza munthu, ndipo atafika m'mudzimo, analephera kuyendetsa bwino komwe anawombana ndi galimotolo
Malemu Keyala amalowera dera la Kapiri kuchoka kwa Kamwendo mu msewu wa Mchinji-Kasungu Emu eitini, atakweza munthu, ndipo atafika m'mudzimo, analephera kuyendetsa bwino komwe anawombana ndi galimotolo
Female
Wofalitsa nkhani za apolisi ku Mchinji a Limbani Mpinganjira wati kutsatira izi, a Keyala anavulala m'mutu ndipo amwalira akulandira thandizo pa chipatala cha Mchinji, pomwe munthu wokwezedwayo wathyoka miyendo
Wofalitsa nkhani za apolisi ku Mchinji a Limbani Mpinganjira wati kutsatira izi, a Keyala anavulala m'mutu ndipo amwalira akulandira thandizo pa chipatala cha Mchinji, pomwe munthu wokwezedwayo wathyoka miyendo
Female
Kafukufuku yemwe bungwe loona zampikisano pamalonda la FCTC lachita waonetsa kuti ochita malonda ena akuphwanya malamulo akamagulitsa sugar
Kafukufuku yemwe bungwe loona zampikisano pamalonda la efisitisi lachita waonetsa kuti ochita malonda ena akuphwanya malamulo akamagulitsa shuga
Female
Kalata yabungweli yomwe wasainila ndi mkulu wake a Lloyds Vincent Nkhoma ena akugulitsa sugar pang'ono pang'ono, pogwiritsa ntchito mitengo yokwera kuyerekeza ndi mtengo oyenera mwa zina
Kalata yabungweli yomwe wasainila ndi mkulu wake a Loidi Vinisenti Nkhoma ena akugulitsa sshuga pang'ono pang'ono, pogwiritsa ntchito mitengo yokwera kuyerekeza ndi mtengo oyenera mwa zina
Female