audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
kuti anthu anayi agwidwa potsatira zipolowezi. A Singanyama ati anthuwa ndi ochokera m'maboma a kummwera kwa dziko lino ndipo maina awo ndi Joe Manda wa zaka 38,Charles Phiri wa zaka 35 | kuti anthu anayi agwidwa potsatira zipolowezi. A Singanyama ati anthuwa ndi ochokera m'maboma a kummwera kwa dziko lino ndipo maina awo ndi Jo Manda wa zaka fete eiti ,Tchalosi Phiri wa zaka Fete faifi | Female | |
Blessings Gawani wa zaka 18 ndi Wabwino Amino wa zaka 30,ndipo onsewa akayankha Milandu yovulaza anthu ndi kuonongetsa katundu ochuluka | Blessings Gawani wa zaka eitini ndi Wabwino Amino wa zaka fete,ndipo onsewa akayankha Milandu yovulaza anthu ndi kuonongetsa katundu ochuluka | Female | |
Bungwe lokonza ndi kulembetsa mayeso mdziko muno la MANEB lati ophunzira 276,052 ndiwo akuyembekezeka kulemba mayeso a Standard 8 a chaka chino | Bungwe lokonza ndi kulembetsa mayeso mdziko muno la MANEBU lati ophunzira thu handede andi sevente sikisi sauzande andi fifite thu ndiwo akuyembekezeka kulemba mayeso a sitandade eiti a chaka chino | Female | |
omwe ayambe lachitatu pa 10 May, 2023. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe bungweli latulutsa lachiwiri pa 9 May | omwe ayambe lachitatu teni meyi twente twente fili. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe bungweli latulutsa lachiwiri pa naini meyi | Female | |
yomwe yati mwa ophunzirawa 134,040 ndi anyamata ndipo 142,012 ndi atsikana | yomwe yati mwa ophunzirawa wani handed andi fetefo sauzande andi fote ndi anyamata ndipo wani handede andi fote thu sauzande andi thwelofu ndi atsikana | Female | |
Kalatayi yati bungweli lakhadzikitsa nambala ya lamya yaulele yomwe ndi 363 yomwe anthu aziyimbira a Maneb akaona mchitidwe uliwonse wachinyengo pa mayesowa | Kalatayi yati bungweli lakhadzikitsa nambala ya lamya yaulele yomwe ndi fili sikisi fili yomwe anthu aziyimbira a Manebu akaona mchitidwe uliwonse wachinyengo pa mayesowa | Female | |
Mwazina chiwerengero cha ophunzira chaka chino ndi chokwera poyerekeza ndi chaka chatha chifukwa chaka chatha ana omwe analembetsa mkaundula olemba mayeso analipo 260,265 | Mwazina chiwerengero cha ophunzira chaka chino ndi chokwera poyerekeza ndi chaka chatha chifukwa chaka chatha ana omwe analembetsa mkaundula olemba mayeso analipo thu handede andi sikisite sauzande thu handede andi sikisite faifi | Female | |
Bwalo lalikulu la milandu ku Zomba lagamula kuti unduna wa maphunziro uzilola ana ama Rasta kuti azilowa mkalasi m' sukulu zonse za boma | Bwalo lalikulu la milandu ku Zomba lagamula kuti unduna wa maphunziro uzilola ana ama Rasita kuti azilowa mkalasi m' sukulu zonse za boma | Female | |
Judge Zione Ntaba yemwe amazenga mlanduwu wati ndi kulakwa kuletsa ana ama Rasta omwe amasunga tsitsi kuti asalowe m' kalasi | Jaji Zione Ntaba yemwe amazenga mlanduwu wati ndi kulakwa kuletsa ana ama Rasita omwe amasunga tsitsi kuti asalowe m' kalasi | Female | |
Khoti lalamulanso kuti loma lilembele kalata sukulu zake zonse pomafika pa 30 june kudziwitsa sukulu iliyonse M'malawi muno kuti sikololedwa kukana mwana wa Rasta kuti asalowe m'kalasi kamba koti sanamete tsitsi | Khoti lalamulanso kuti loma lilembele kalata sukulu zake zonse pomafika pa fete juni kudziwitsa sukulu iliyonse M'malawi muno kuti sikololedwa kukana mwana wa Rasita kuti asalowe m'kalasi kamba koti sanamete tsitsi | Female | |
Kumbali yake yemwe amaimilila mlandu kwa ana ama Rasta, Chikondi Chijoza wati ndi okhutira ndi chigamulocho | Kumbali yake yemwe amaimilila mlandu kwa ana ama Rasita, Chikondi Chijoza wati ndi okhutira ndi chigamulocho | Female | |
ndipo khoti linagwirizana kuti zinali zolakwika kuletsa ana ama Rasta kuti asalowe m'kalasi kamba ka tsitsi lawo | ndipo khoti linagwirizana kuti zinali zolakwika kuletsa ana ama Rasita kuti asalowe m'kalasi kamba ka tsitsi lawo | Female | |
Gulu lina lotchedwa Dzuka Malawi lati likufuna Atupele Muluzi kuti atsogolere chipani cha United Democratic Front (UDF) | Gulu lina lotchedwa Dzuka Malawi lati likufuna Atupele Muluzi kuti atsogolere chipani cha yunaitedi demokilatiki fulanti (yudiefu) | Female | |
komanso adzaimire mpando wa mtsogoleri wa dziko pa chisakho cha 2025. Poyakhula kwa atolakhani Msungichuma wa Dzuka Malawi, Isaac Lalama | komanso adzaimire mpando wa mtsogoleri wa dziko pa chisakho cha twente twente faifi. Poyakhula kwa atolakhani Msungichuma wa Dzuka Malawi, Iaizeki Lalama | Female | |
wati a Muluzi ndioyenera kuti atsogolere chipanichi kamba koti alibe mbiri ina iliyonse yolakwika | wati a Muluzi ndioyenera kuti atsogolere chipanichi kamba koti alibe mbiri ina iliyonse yolakwika | Female | |
Iwo atinso a Muluzi akhala akugwira ntchito ya ma unduna osiyanasiya zomwe zikupeleka chithuzi thunzi kuti ali ndi ukadaulo pa ndale komanso kayendetsedwe ka boma | Iwo atinso a Muluzi akhala akugwira ntchito ya ma unduna osiyanasiya zomwe zikupeleka chithuzi thunzi kuti ali ndi ukadaulo pa ndale komanso kayendetsedwe ka boma | Female | |
Gululi lili ndi mamembala opitilila 1000 mdziko muno. Mfumu yayikulu Malemia ya boma la Nsanje yadandaula kuti akulu akulu ogwira ntchito mma ofesi ena a boma | Gululi lili ndi mamembala opitilila wani sauzande mdziko muno. Mfumu yayikulu Malemya ya boma la Nsanje yadandaula kuti akulu akulu ogwira ntchito mma ofesi ena a boma | Female | |
ndiomwe akuchedwesa ntchito yosamusa anthu omwe adakhuzika ndi Namondwe wa Freddy kuti apite madera ena. A Malemia ati ngakhale anasatira dongosolo lolemba kalata ku Ofesi ya boma la Nsanje | ndiomwe akuchedwesa ntchito yosamusa anthu omwe adakhuzika ndi Namondwe wa Fulede kuti apite madera ena. A Malemya ati ngakhale anasatira dongosolo lolemba kalata ku Ofesi ya boma la Nsanje | Female | |
palibe chomwe chikuchitika. Iwo alakhula izi pomwe bungwe la Southern Region Water Board limapereka thandizo losiyana siyana kwa maanja okwana 450 omwe akukhala pa msasa wa Mota-Engil | palibe chomwe chikuchitika. Iwo alakhula izi pomwe bungwe la sauveni lijoni wota bodi limapereka thandizo losiyana siyana kwa maanja okwana fo handiledi andi fifite omwe akukhala pa msasa wa Mota-Engelo | Female | |
Ndipo bwanamkubwa wa bomali a Dominic Mwandira avomereza kuti ntchito yosamutsa anthuwa yachedwa kamba koti panalinso mudzi wina wa Mambundu womwe ufunikanso kuti usamuke | Ndipo bwanamkubwa wa bomali a Dominiki Mwandira avomereza kuti ntchito yosamutsa anthuwa yachedwa kamba koti panalinso mudzi wina wa Mambundu womwe ufunikanso kuti usamuke | Female | |
Ndipo wa pa mpando wa bungwe la Southern region water board, Brown Mpinganjira ati agwiritsa ntchito chuma cha bungweli komanso ma Directors adasokherana ndikugula katundu osiyana siyana | Ndipo wa pa mpando wa bungwe la sauveni lijoni wota bodi, Brown Mpinganjira ati agwiritsa ntchito chuma cha bungweli komanso ma Dailekitazi adasokherana ndikugula katundu osiyana siyana | Female | |
kuti athandize anthu omwe anakhunzidwa ndi Namondwe wa Freddy .Thandizoli apereka ma Boma a Mulanje ndi Nsanje ndipo ndi la ndalama zokwana 25 Million | kuti athandize anthu omwe anakhunzidwa ndi Namondwe wa Fulede .Thandizoli apereka ma Boma a Mulanje ndi Nsanje ndipo ndi la ndalama zokwana twente faifi miliyoni | Female | |
Bambo wina yemwe dzina lake ndi Osman Makwinja wathawa atapha mwana wake omupeza kaamba koti mwanayo analetsetsa ndewu yapakati pa mayi ake ndi bambo ake omupezawo | Bambo wina yemwe dzina lake ndi Osimani Makwinja wathawa atapha mwana wake omupeza kaamba koti mwanayo analetsetsa ndewu yapakati pa mayi ake ndi bambo ake omupezawo | Female | |
pa 16 April, 2023 m'boma la Thyolo. Wachiwiri kwa wofalitsa nkhani zapolisi ku Thyolo Sergeant Rabecca Kashoti | pa sikisitini epulo twente twente fili m'boma la Thyolo. Wachiwiri kwa wofalitsa nkhani zapolisi ku Thyolo Sajenti Rabeka Kashoti | Female | |
wauza Ufulu FM kuti mwana ophedwayu dzina lake ndi Evance Mpaso, wa zaka 17 zakubadwa, wa mmudzi wa Sunganani, mfumu yaikulu Chimaliro m'boma lomwelo la Thyolo | wauza Ufulu efuemu kuti mwana ophedwayu dzina lake ndi Evansi Mpaso, wa zaka seventini zakubadwa, wa mmudzi wa Sunganani, mfumu yaikulu Chimaliro m'boma lomwelo la Thyolo | Female | |
A Kashoti ati mmawa wa Lamulungu pa 16 April, bambo ndi mayi Makwinja anasemphana chichewa kotero ndewu inayambika | A Kashoti ati mmawa wa Lamulungu pa sikisitini epulo , bambo ndi mayi Makwinja anasemphana chichewa kotero ndewu inayambika | Female | |
mwana ataona izi analetsetsa awiriwo koma izi sizinakondweretse bamboyo kotero anatenga mpeni ndi kubaya mwanayo pachifuwa | mwana ataona izi analetsetsa awiriwo koma izi sizinakondweretse bamboyo kotero anatenga mpeni ndi kubaya mwanayo pachifuwa | Female | |
Zitachitika izi mayi amwanayu anathamangira naye ku chipatala chaching'ono cha Chisoka komwe achipatala anatsimikiza kuti mwanayo wamwalira | Zitachitika izi mayi amwanayu anathamangira naye ku chipatala chaching'ono cha Chisoka komwe achipatala anatsimikiza kuti mwanayo wamwalira | Female | |
Pakadali pano apolisi m'bomalo akusakasaka mkuluyu kuti akayankhe mlandu wakupha. Unduna wa zaulimi wati ukhala tcheru | Pakadali pano apolisi m'bomalo akusakasaka mkuluyu kuti akayankhe mlandu wakupha. Unduna wa zaulimi wati ukhala tcheru | Female | |
pofuna kuonetsetsa kuti malonda a fodya a chaka chino ayende molongosoka komanso mokomera alimi mdziko muno. Mlembi wamkulu ku unduna oona zaulimi, Dixie Kampani | pofuna kuonetsetsa kuti malonda a fodya a chaka chino ayende molongosoka komanso mokomera alimi mdziko muno. Mlembi wamkulu ku unduna oona zaulimi, Dikisi Kampani | Female | |
wayankhula izi lolemba pomwe amatsegulira msika wa fodya wa Limbe Auction Floors ku Blantyre. A Kampani mwa zina ati unduna wao | wayankhula izi lolemba pomwe amatsegulira msika wa fodya wa Limbe okoshini fulozi ku Bulantaya. A Kampani mwa zina ati unduna wao | Female | |
wauza adindo oyendetsa msika wa fodya kuti adzipereka malipoti a mmene malonda a fodya akuyendera sabata iliyonse ndi cholinga choti azitha kutsatira bwino zinthu | wauza adindo oyendetsa msika wa fodya kuti adzipereka malipoti a mmene malonda a fodya akuyendera sabata iliyonse ndi cholinga choti azitha kutsatira bwino zinthu | Female | |
Iwo apemphanso alimi a fodya kuti azitsogoza zokambirana pomwe ali ndi nkhawa mmalo moyambitsa mpungwepungwe zomwe ati zimasokoneza malondawa | Iwo apemphanso alimi a fodya kuti azitsogoza zokambirana pomwe ali ndi nkhawa mmalo moyambitsa mpungwepungwe zomwe ati zimasokoneza malondawa | Female | |
M'mau ake, wapampando wa board ya bungwe lomwe limayendetsa malonda a fodya la Tobbaco Commission, Dr Godfrey Chapola wati chaka chino pa msika pali fodya olemera makilogalamu 126 million | M'mau ake, wapampando wa bodi ya bungwe lomwe limayendetsa malonda a fodya la Tobako komishoni, Dokota Godifule Chapola wati chaka chino pa msika pali fodya olemera makilogalamu wani handiledi andi twente sikisi miliyoni | Female | |
yemwe ndi ochuluka kuposa makilogalamu okwana 85 million a fodya chaka chatha. A Chapola ati fodya wachuluka chotere kaamba ka mitengo yabwino ya fodya pa msika wa Chaka chatha | yemwe ndi ochuluka kuposa makilogalamu okwana eite faifi miliyoni a fodya chaka chatha. A Chapola ati fodya wachuluka chotere kaamba ka mitengo yabwino ya fodya pa msika wa Chaka chatha | Female | |
kampani zogula fodya zinapereka zipangizo moyenera komanso kwabwera alimi atsopano. Naye, wapampando wa board ya AHL Group, Dr Jerome Nkhoma | kampani zogula fodya zinapereka zipangizo moyenera komanso kwabwera alimi atsopano. Naye, wapampando wa bodi ya e etchi elo gulupu, Dokota Jerome Nkhoma | Female | |
watsimikizira alimi a fodya kuti awonesetsa kuti alimi akugulitsa fodya wao pa mitengo yabwino kuti apindule. Msika wa fodya wa Limbe Auction Floors | watsimikizira alimi a fodya kuti awonesetsa kuti alimi akugulitsa fodya wao pa mitengo yabwino kuti apindule. Msika wa fodya wa Limbe okoshoni fulozi | Female | |
anautsegulira mchaka Cha 1936 ndipo ndi msika oyamba wa fodya kutsegulidwa mdziko muno. Bungwe lothandiza anthu ovutika la Chikondi Foundation | anautsegulira mchaka Cha naintini fete sikisi ndipo ndi msika oyamba wa fodya kutsegulidwa mdziko muno. Bungwe lothandiza anthu ovutika la Chikondi Faundeshoni | Female | |
lapempha boma kuti likhadzikitse ndondomeko zomwe zilimbikitse ophunzira omwe anakhudzidwa ndi Namondwe wa Freddy kuti adzachite bwino pa mayeso a boma omwe ayambe mwezi wa mawa | lapempha boma kuti likhadzikitse ndondomeko zomwe zilimbikitse ophunzira omwe anakhudzidwa ndi Namondwe wa Fulede kuti adzachite bwino pa mayeso a boma omwe ayambe mwezi wa mawa | Female | |
Mkulu wa bungweli Chikondi Kuphata ndiye wanena izi pomwe amapereka thandizo kwa ophunzira a Standard 8 omwe akuphunzira komanso kukhala pa msasa wa Mpoto m'boma la Phalombe | Mkulu wa bungweli Chikondi Kuphata ndiye wanena izi pomwe amapereka thandizo kwa ophunzira a sitandade eiti omwe akuphunzira komanso kukhala pa msasa wa Mpoto m'boma la Phalombe | Female | |
Atalandira nthandizoli, mmodzi wa ophunzira Brenda Chiona wati iye pamodzi ndi anzake ali pachiopsezo chosachita bwino mayeso awo a Maneb | Atalandira nthandizoli, mmodzi wa ophunzira Bulenda Chiona wati iye pamodzi ndi anzake ali pachiopsezo chosachita bwino mayeso awo a Manebu | Female | |
kamba koti pamsasa pomwe akukhala pakumakhala pokhoso lochuluka kotero akulephera kuwerenga | kamba koti pamsasa pomwe akukhala pakumakhala pokhoso lochuluka kotero akulephera kuwerenga | Female | |
Katundu yemwe bungwe la Chikondi Foundation lapereka kwa ophunzirawa ndi monga zovala, sopo ndi ma pad, mwazina | Katundu yemwe bungwe la Chikondi Faundeshoni lapereka kwa ophunzirawa ndi monga zovala, sopo ndi ma padi, mwazina | Female | |
Adindo omwe angosankhidwa kumene kuti atsogolere ochemelera atimu ya Mighty Mukuru Wanderers muchigawo chapakati, akumana koyamba ndikukambirana za momwe angagwilire ntchito limodzi zotukura timu yawo | Adindo omwe angosankhidwa kumene kuti atsogolere ochemelera atimu ya Maite Mukuru Wandilazi muchigawo chapakati, akumana koyamba ndikukambirana za momwe angagwilire ntchito limodzi zotukura timu yawo | Female | |
Mkumanowu wachitika ku Crossroads Hotel ndipo adindowa agwilizana kuti ayendere Pamodzi ndipo kusemphana komwe kunalipo m'mbuyomu kumbali ya ochemelerawa kuthe | Mkumanowu wachitika ku khulosilodzi hotelo ndipo adindowa agwilizana kuti ayendere Pamodzi ndipo kusemphana komwe kunalipo m'mbuyomu kumbali ya ochemelerawa kuthe | Female | |
Adindo omwe asankhidwawa, m'mbuyomu anali muma camp osiyanasiyana zomwe zimapangitsa kuti pakhale kukokanakokana poti aliyense amafuna utsogoleri | Adindo omwe asankhidwawa, m'mbuyomu anali muma kampu osiyanasiyana zomwe zimapangitsa kuti pakhale kukokanakokana poti aliyense amafuna utsogoleri | Female | |
Nkhalapampando yemwe wasankhidwa kuti atsogolere ochemelera atimu ya manoma muchigawo chapakati Rodreck Chitedze, wati committe yawo iyesesa kuti ikhale yachitsanzo muzigawo zonse | Nkhalapampando yemwe wasankhidwa kuti atsogolere ochemelera atimu ya manoma muchigawo chapakati Rodileki Chitedze, wati komiti yawo iyesesa kuti ikhale yachitsanzo muzigawo zonse | Female | |
kuti ena azitengera iwo popewa kupanga zinthu zomwe zingawagawanise. Ndipo mumawu ake yemwe wasankhidwa kukhala mlembi wamkulu Bishop Chimwenje | kuti ena azitengera iwo popewa kupanga zinthu zomwe zingawagawanise. Ndipo mumawu ake yemwe wasankhidwa kukhala mlembi wamkulu Bishopu Chimwenje | Female | |
wapempha ochemelera atimuyi ochokera muma zone kuti lachiwili akakumane ku crown lodge masana kuti akakambirane mene ayendetsere timu yawoi limodzi | wapempha ochemelera atimuyi ochokera muma zone kuti lachiwili akakumane ku kolawuni loji masana kuti akakambirane mene ayendetsere timu yawoi limodzi | Female | |
Apolisi m'boma la Mulanje akusunga mchitolokosi mtsikana wa zaka 17, Chrissy Katuli kaamba kopha mchimwene wake Innocent Mandela wa zaka 32 pomumenya mmutu ndi musi | Apolisi m'boma la Mulanje akusunga mchitolokosi mtsikana wa zaka seventini, khilise Katuli kaamba kopha mchimwene wake Inosenti Mandela wa zaka fete thu pomumenya mmutu ndi musi | Female | |
Wofalitsa nkhani za apolisi m'bomalo Sergeant Innocent Moses wati izi zachitika Lamulungu pa 2 April, 2023 mmudzi mwa Ngolowera mfumu yaikulu Chikumbu | Wofalitsa nkhani za apolisi m'bomalo sajenti inosenti mozesi wati izi zachitika Lamulungu pa thu epulo twente twente fili mmudzi mwa Ngolowera mfumu yaikulu Chikumbu | Female | |
A Moses ati a malume a awiriwa anauza apolisi kuti Chrissy ndi Innocent anakangana pa nkhani yokhudza malalanje zomwe zinayambitsa ndeu pakati pawo | A Mozesi ati a malume a awiriwa anauza apolisi kuti khiilise ndi Inosenti anakangana pa nkhani yokhudza malalanje zomwe zinayambitsa ndeu pakati pawo | Female | |
Mphamvu zitamchepera, Chrissy anatenga musi ndi kummenya nawo m'bale wake mmutu. Izi zitachitika nkhaniyi inabisidwa mpaka Lolemba pa 3 April pomwe omenyedwayu wamwalira | Mphamvu zitamchepera, Khilise anatenga musi ndi kummenya nawo m'bale wake mmutu. Izi zitachitika nkhaniyi inabisidwa mpaka Lolemba pa fili Epulo pomwe omenyedwayu wamwalira | Female | |
Atero Malume a awiriwa. Ogwira ntchito zaumoyo pa chipatala cha Mulanje Mission atapima thupilo apeza kuti Innocent wamwalira kaamba kovulala kwambiri mmutu | Atero Malume a awiriwa. Ogwira ntchito zaumoyo pa chipatala cha Mulanje Mishoni atapima thupilo apeza kuti Inosenti wamwalira kaamba kovulala kwambiri mmutu | Female | |
Ndipo apolisi ati Chrissy akaonekera ku bwalo la mlandu posachedwapa kuti akayankhe mlandu. Wachiwiri kwa Speaker wa Nyumba ya Malamulo, Madalitso Kazombo pa modzi ndi bungwe la Water Aid | Ndipo apolisi ati khilise akaonekera ku bwalo la mlandu posachedwapa kuti akayankhe mlandu. Wachiwiri kwa Sipika wa Nyumba ya Malamulo, Madalitso Kazombo pa modzi ndi bungwe la wota edi | Female | |
apereka katundu osiyana siyana kwa anthu omwe anakhunzidwa ndi Namondwe wa Freddy m'boma la Zomba. Mawanja okwana 150 omwe akukhala pa sukulu ya pulaimale ya Namisonju | apereka katundu osiyana siyana kwa anthu omwe anakhunzidwa ndi Namondwe wa Fulede m'boma la Zomba. Mawanja okwana wani handede andi fifite omwe akukhala pa sukulu ya pulaimale ya Namisonju | Female | |
kwa mfumu yayikulu Mwambo ndi omwe alandira nawo katunduyu. Wina mwa katunduyu ndi Ufa, Sugar, Mchere, Soap, Mbale ndi zina za ndalama yokwana K53 million | kwa mfumu yayikulu Mwambo ndi omwe alandira nawo katunduyu. Wina mwa katunduyu ndi Ufa, Shuga, Mchere, Sopo, Mbale ndi zina za ndalama yokwana fifite fili miliyoni kwacha | Female | |
Katunduyu akuyembekezeka kuperekedwanso m'maboma a Mangochi, Machinga ndi madera ena a Zomba. Ophunzira wa chaka chachiwiri pa sukulu ya ukachenjede ya Unima ku Zomba | Katunduyu akuyembekezeka kuperekedwanso m'maboma a Mangochi, Machinga ndi madera ena a Zomba. Ophunzira wa chaka chachiwiri pa sukulu ya ukachenjede ya yunima ku Zomba | Female | |
wapezeka atazimangilira ku denga kwa chipinda chake chogona usiku wathawu. Mneneri wa Polisi ku Zomba, Patricia Supiliano | wapezeka atazimangilira ku denga kwa chipinda chake chogona usiku wathawu. Mneneri wa Polisi ku Zomba, Patilisha Supiliyano | Female | |
watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti dzina la ophunzirayu ndi Ipen Chimphanga wa zaka 25 zakubadwa | watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti dzina la ophunzirayu ndi ayipeni Chimphanga wa zaka twente faifi zakubadwa | Female | |
Iwo ati anzake omwe amabwera kuchokera kowerenga anampeza mnyamatayu atazimangilira ku denga. Padakali pano, thupi la malemuwa lili ku chipatala chachikulu cha Zomba kuti alipime | Iwo ati anzake omwe amabwera kuchokera kowerenga anampeza mnyamatayu atazimangilira ku denga. Padakali pano, thupi la malemuwa lili ku chipatala chachikulu cha Zomba kuti alipime | Female | |
Ipen Chimphanga amachokera m'mudzi mwa Kalilima, m’mudzi wa Kalalima mfumu yaikulu Chakhadza m'boma la Dowa | ayipeni Chimphanga amachokera m'mudzi mwa Kalilima, m’mudzi wa Kalalima mfumu yaikulu Chakhadza m'boma la Dowa | Female | |
Bungwe la Sight Saver lapereka upangiri kwa mabungwe okhudzidwa polimbikitsa anthu a ulumari powaunikira kuti ali ndi kuthekera kutukula chuma cha dziko lino | Bungwe la saiti seva lapereka upangiri kwa mabungwe okhudzidwa polimbikitsa anthu a ulumari powaunikira kuti ali ndi kuthekera kutukula chuma cha dziko lino | Female | |
Polakhula la Chitatu pa mkumano womwe bungweli linakonza mzinda wa Blantyre, mkulu wa bungwe la Sight Saver Bright Chiwaula wati anthu aulumali nawo ali ndikuthekera kutukula dziko lino pa chuma | Polakhula la Chitatu pa mkumano womwe bungweli linakonza mzinda wa Bulantaya, mkulu wa bungwe la saiti seva Bulaiti Chiwaula wati anthu aulumali nawo ali ndikuthekera kutukula dziko lino pa chuma | Female | |
kutero adzipatsidwa mwayi wopeza ngongole zopangira ma buzinesi osiyanasiyana. Anthu ulumali amasiyidwa kumbali poganiza kuti kwawo ndi kupephetsa m'matauni | kutero adzipatsidwa mwayi wopeza ngongole zopangira ma buzinesi osiyanasiyana. Anthu ulumali amasiyidwa kumbali poganiza kuti kwawo ndi kupephetsa m'matauni | Female | |
omwe ndi maganizo olakwika popeza kuti nawo atha kutukula dziko lino anatero a Chiwaula. A Chiwaula ati anthu okwana 480 a m'maboma a Dedza ndi Machinga | omwe ndi maganizo olakwika popeza kuti nawo atha kutukula dziko lino anatero a Chiwaula. A Chiwaula ati anthu okwana folo handiledi andi aite a m'maboma a Dedza ndi Machinga | Female | |
omwe ali ndi ulumali tsopano ayamba kupatsidwa mwayi opeza nawo ngongole ku mabanki ndi mabungwe kuti athandizire pochita ma bizinesi osiyanasiyana kuphatikizapo a ulimi | omwe ali ndi ulumali tsopano ayamba kupatsidwa mwayi opeza nawo ngongole ku mabanki ndi mabungwe kuti athandizire pochita ma bizinesi osiyanasiyana kuphatikizapo a ulimi | Female | |
Ena mwa mabungwe omwe anali nawo pa mkumanowu ndi monga Malawi Union for the Blind, FEDOMA komanso Visual Hearing Empowerment Membership Association of Malawi | Ena mwa mabungwe omwe anali nawo pa mkumanowu ndi monga Malawi yuniyoni fo ve bulaindi, FEDOMA komanso vizyo hiyeling’I impawamenti membashipi ofu Malawi | Female | |
M'mawu ake, mkulu wogwilizira bungwe la FEDOMA Simon Munde ati ndiwokondwa ndi dongosololi ndipo kuti angwiritsa ntchito mwayiwu | M'mawu ake, mkulu wogwilizira bungwe la FEDOMA Simoni Munde ati ndiwokondwa ndi dongosololi ndipo kuti angwiritsa ntchito mwayiwu | Female | |
Galimoto yayikulu yomwe idanyamula Chimanga kuti ikapeleke kwa anthu omwe anakhunzidwa ndi Namondwe wa Freddy, yachita ngozi nsewu wa Nayuchi boma la Machinga | Galimoto yayikulu yomwe idanyamula Chimanga kuti ikapeleke kwa anthu omwe anakhunzidwa ndi Namondwe wa Fulede, yachita ngozi nsewu wa Nayuchi boma la Machinga | Female | |
Galimotoyi ndi yomwe ikuganizilidwa kuti idazembesedwa ndi Councillor Alexander Cosmas yemwenso anali wa pa mpando owona ngozi zogwa mwadzidzidzi m'boma la Machinga ndipo anamangidwa Loweruka lapitali | Galimotoyi ndi yomwe ikuganizilidwa kuti idazembesedwa ndi khansala alekizanda kosimasi yemwenso anali wa pa mpando owona ngozi zogwa mwadzidzidzi m'boma la Machinga ndipo anamangidwa Loweruka lapitali | Female | |
Mneneri wa nkhonsolo ya boma la Machinga, Martin Chiwanda watsimikiza za ngoziyi poyakhula ndi Ufulu FM | Mneneri wa nkhonsolo ya boma la Machinga, Matini Chiwanda watsimikiza za ngoziyi poyakhula ndi Ufulu efuemu | Female | |
Ndipo ati pakadali pano nkhonsolo yawo pamodzi ndi a polisi afika ku malowo kuti akateteze Chimangacho | Ndipo ati pakadali pano nkhonsolo yawo pamodzi ndi a polisi afika ku malowo kuti akateteze Chimangacho | Female | |
Ndipo zadziwika kuti palibe yemwe wafa pa ngoziyi. Padakali galimoto lina lafika pa malopo kuti linyamule chimangacho | Ndipo zadziwika kuti palibe yemwe wafa pa ngoziyi. Padakali galimoto lina lafika pa malopo kuti linyamule chimangacho | Female | |
A polisi a ku Liwonde amanga Alexander Cosmas wapa mpando owona Ngozi Zogwa Mwadzidzi m'boma la Machinga | A polisi a ku Liwonde amanga elekizanda kosimasi wapa mpando owona Ngozi Zogwa Mwadzidzi m'boma la Machinga | Female | |
powaganizira kuti amazembetsa thandizo la katundu wa anthu amene akukhunzidwa ndi Namondwe wa Freddy. Mkulu wa Polisi ku Liwonde a Ulemu Kalua atsimikiza zakumangidwa kwa a Cosmas | powaganizira kuti amazembetsa thandizo la katundu wa anthu amene akukhunzidwa ndi Namondwe wa Fulede. Mkulu wa Polisi ku Liwonde a Ulemu Kaluwa atsimikiza zakumangidwa kwa a Kosimasi | Female | |
Koma iwo ati kafukufuku adakali mkati pa nkhaniyi. Mpingo wa katolika wati uli ndi chiyembekezo kuti Banki yawo ya tsopano ya Centenary ithandiza kukweza miyoyo ya anthu ovutika mdziko muno | Koma iwo ati kafukufuku adakali mkati pa nkhaniyi. Mpingo wa katolika wati uli ndi chiyembekezo kuti Banki yawo ya tsopano ya Centenale ithandiza kukweza miyoyo ya anthu ovutika mdziko muno | Female | |
Archbishop Desmond Tambala wa Lilongwe Diocese ndiyemwe walakhula Izi pa mwambo wotsekulira bankiyi lachitatu ku Lilongwe | Arkibishopu Dezimondi Tambala wa Lilongwe Dayosisi ndiyemwe walakhula Izi pa mwambo wotsekulira bankiyi lachitatu ku Lilongwe | Female | |
Ndipo wachiwiri kwa Governor wa Banki yayikulu mdziko muno a William Matambo ati ali ndi chiyembekezo kuti ntchito za bankiyi zithandiza pa chitukuko ndi kukweza chuma cha dziko lino | Ndipo wachiwiri kwa Gavana wa Banki yayikulu mdziko muno a Wiliyamu Matambo ati ali ndi chiyembekezo kuti ntchito za bankiyi zithandiza pa chitukuko ndi kukweza chuma cha dziko lino | Female | |
Matambo atinso aonetsetsa kuti ntchito za ma Banki zikuyenda bwino mdziko muno. Anthu okhala pa msasa wa Mthuruwe primary school m'boma la Mulanje adandaula ndi kuchepa kwa zimbudzi pa sukuluyi | Matambo atinso aonetsetsa kuti ntchito za ma Banki zikuyenda bwino mdziko muno. Anthu okhala pa msasa wa Mthuruwe pulaimale sukulu m'boma la Mulanje adandaula ndi kuchepa kwa zimbudzi pa sukuluyi | Female | |
zomwe ati zikupereka chiopsezo chodwala nthenda zodza kaamba kosowa ukhondo pa malopa. Mfumu Kamoto yochokera mdera la mfumu yaikulu Mkanda yanena izi pomwe amalandira thandizo | zomwe ati zikupereka chiopsezo chodwala nthenda zodza kaamba kosowa ukhondo pa malopa. Mfumu Kamoto yochokera mdera la mfumu yaikulu Mkanda yanena izi pomwe amalandira thandizo | Female | |
kuchokera ku nthambi ya National Water Resources Authority (NWRA). Mfumuyi yapempha anthu akufuna kwabwino kuti awathandize | kuchokera ku nthambi ya Neshono wota lisosezi ofolite (Eni dabiliyu alae) Mfumuyi yapempha anthu akufuna kwabwino kuti awathandize | Female | |
powamangira zimbudzi zabwino kuti apewe matenda monga otsekula mmimba ndi Cholera | powamangira zimbudzi zabwino kuti apewe matenda monga otsekula mmimba ndi Cholera | Female | |
Galimoto zodzera msewu wa Zomba-Liwonde zikulephera kudutsa pa mlatho wa Mafufuni ku Songani kamba ka Bus yomwe yakakamila pa malopo | Galimoto zodzera msewu wa Zomba-Liwonde zikulephera kudutsa pa mlatho wa Mafufuni ku Songani kamba ka Basi yomwe yakakamila pa malopo | Female | |
Pakadali pano galimoto zikudikira kuti Bus yi mwina ichoka. Izi zachitika Usiku pomwe Bus yi yakakamila pa mlathowo, pomwe mvula yakhala ikugwa usiku wonse ku Zomba | Pakadali pano galimoto zikudikira kuti Basi yi mwina ichoka. Izi zachitika Usiku pomwe Basi yi yakakamila pa mlathowo, pomwe mvula yakhala ikugwa usiku wonse ku Zomba | Female | |
Galimoto zina zayamba kale kuzungulira ndi kudutsa msewu wa Zalewa. Nyanja ya Chilwa ku Zomba yadzadza pomwe madzi akusefukira kufika midzi yoyandikana | Galimoto zina zayamba kale kuzungulira ndi kudutsa msewu wa Zalewa. Nyanja ya Chilwa ku Zomba yadzadza pomwe madzi akusefukira kufika midzi yoyandikana | Female | |
Izi zikudza kutsatira kwa mvula ya mphamvu yomwe yagwa kamba ka Namondwe wa Freddy. A Fanuel Sadick omwe amakhala kuderali | Izi zikudza kutsatira kwa mvula ya mphamvu yomwe yagwa kamba ka Namondwe wa Fulede. A Fanuwelo Sadiki omwe amakhala kuderali | Female | |
auza Ufulu FM online kuti madzi afika midzi yoyandikila doko la Kachulu ndipo anthu akusamukira ku madera ena | auza Ufulu efuemu onilayini kuti madzi afika midzi yoyandikila doko la Kachulu ndipo anthu akusamukira ku madera ena | Female | |
Chiwerengero cha anthu omwe ataya moyo kamba ka ngozi za kusefukira kwa thope ndi madzi zomwe zadza ndi Namondwe wa Freddy, chafika pa 438 tsopano, kuchoka pa 326 | Chiwerengero cha anthu omwe ataya moyo kamba ka ngozi za kusefukira kwa thope ndi madzi zomwe zadza ndi Namondwe wa Fulede, chafika pa folo handiledi andi fete eiti tsopano, kuchoka pa fili handiledi andi twente sikisi | Female | |
Malingana ndi kalata yomwe atulusa a nthambi yowona za Ngozi zogwa mwadzizi M'dziko muno. Anthu oposa 345,000 akusowa pokhala | Malingana ndi kalata yomwe atulusa a nthambi yowona za Ngozi zogwa mwadzizi M'dziko muno. Anthu oposa fili handiledi andi fote faifi sauzande akusowa pokhala | Female | |
ndipo pakadali pano Misasa yokwana 505 yakhazikisidwa. Anthu 282 akusowa ndipo anthu oposa 900 ndi ovulala | ndipo pakadali pano Misasa yokwana faifi handiledi andi faifi yakhazikisidwa. Anthu thu handiledi andi eite thu akusowa ndipo anthu oposa naini handiledi ndi ovulala | Female | |
Bungwe logawa madzi la Southern Region Water Board lati ndi lokhuzidwa kwambiri ndi mmene Namondwe wa Freddy wakhudzira ku chigawo cha kumwera | Bungwe logawa madzi la sauveni lijoni wota bodi lati ndi lokhuzidwa kwambiri ndi mmene Namondwe wa Fulede wakhudzira ku chigawo cha kumwera | Female | |
Mneneri wa bungweli, Ritta Makwangwala, wati Namondwe wa Freddy wakokolola ena mwa mapaipi omwe amatengelako madzi | Mneneri wa bungweli, Rita Makwangwala, wati Namondwe wa Fulede wakokolola ena mwa mapaipi omwe amatengelako madzi | Female | |
komanso mapaipi ena omwe amatenga madzi kupititsa mmakomo mwa makasitomala awo. Iwo ati ogwira ntchito ku bungwe lawo akuyesetsa kukonza mapaipi omwe aonongeka | komanso mapaipi ena omwe amatenga madzi kupititsa mmakomo mwa makasitomala awo. Iwo ati ogwira ntchito ku bungwe lawo akuyesetsa kukonza mapaipi omwe aonongeka | Female | |
pofuna anthu apitilire kumwa madzi otetezeka. Ndipo padakali pano, bungweli latumiza magalimoto opeleka madzi( water Bowsers) m'madera omwe akhunzidwa maka mu zipatala | pofuna anthu apitilire kumwa madzi otetezeka. Ndipo padakali pano, bungweli latumiza magalimoto opeleka madzi( water Bauzazi) m'madera omwe akhunzidwa maka mu zipatala | Female | |
Gulu la Sound Addicts lomwe lakonza mwambo wa mayimbidwe wa Ku Mingoli Bash womwe uzachitike pa 22 July ku Lilongwe Golf Club, lati lakonza izi ndi cholinga choti aMalawi azasangalale | Gulu la saundi adikitsi lomwe lakonza mwambo wa mayimbidwe wa Ku Mingoli Bashi womwe uzachitike pa twente thu julayi ku Lilongwe gofu kilabu, lati lakonza izi ndi cholinga choti aMalawi azasangalale | Female | |
Mmodzi mwa akuluakulu a Sound Addicts Shadreck Kalukusha walankhula izi pa msonkhano wa atolankhani lachitatu ku Lilongwe | Mmodzi mwa akuluakulu a saundi adikitsi shadileki Kalukusha walankhula izi pa msonkhano wa atolankhani lachitatu ku Lilongwe | Female | |
A Kalukusha atinso padakali pano ayamba kale kugulitsa ma ticket ndipo akhala akukweza mtengo pa sabata zitatu pomwe akuyandika ku mwambowo | A Kalukusha atinso padakali pano ayamba kale kugulitsa ma tiketi ndipo akhala akukweza mtengo pa sabata zitatu pomwe akuyandika ku mwambowo | Female | |
Ndipo kazembe wa mwambo wa Ku Mingoli pa ntchito za msangulutso Felistus Nyauyu Ngwira | Ndipo kazembe wa mwambo wa Ku Mingoli pa ntchito za msangulutso Felisitasi Nyauyu Ngwira | Female | |
akufotokoza kuti oyimba okwana anayi akunja ndi oposa khumi amdziko muno omwe azasangalase anthu pa 22 July | akufotokoza kuti oyimba okwana anayi akunja ndi oposa khumi amdziko muno omwe azasangalase anthu pa twente thu julayi | Female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.