audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
zomwe zadakwitsa makhansala. A Jana atiuza kuti a Mayor ndi wachiwiri wawo adapita ku Lilongwe kukaonera masewero ampira a Chikho Cha FDH Intercity Mayor's Trophy | zomwe zadakwitsa makhansala. A Jana atiuza kuti a Meya ndi wachiwiri wawo adapita ku Lilongwe kukaonera masewero ampira a Chikho Cha Efudietchi intasite meyazi thilofe | Female | |
Kulepheleka kwa Full Council Meeting kwatikhuza chifkwa timayenera kuti tikambirane ntchito zachitukuko monga, zamisewu zomwe zaima, komanso kuti Stadium ya Zomba sikutha chifukwa chani | Kulepheleka kwa Fukhanso miting’i kwatikhuza chifkwa timayenera kuti tikambirane ntchito zachitukuko monga, zamisewu zomwe zaima, komanso kuti Sitediyamu ya Zomba sikutha chifukwa chani | Female | |
adatero a Jana. Ndipo m'modzi mwa amene amaimilila anthu ochita malonda a Dan Phiri ati kulepheleka kwa full Council meeting zawakhudza ndipo ngati ma Interest Group | adatero a Jana. Ndipo m'modzi mwa amene amaimilila anthu ochita malonda a Dani Phiri ati kulepheleka kwa Fukhanso miting’i zawakhudza ndipo ngati ma intilesiti gulupu | Female | |
ambiri amachita kulandira ma kalata oti apite tsiku lakuti lakuti zomwe nawonso anadwabwa akuuzidwa kuti full council meeting yalepheleka kungouzidwa atafika kale | ambiri amachita kulandira ma kalata oti apite tsiku lakuti lakuti zomwe nawonso anadwabwa akuuzidwa kuti Fukhanso miting’i yalepheleka kungouzidwa atafika kale | Female | |
Koma Mayor wa mu mzindawu a Davie Maunde ati kunalibe full council meeting koma unali msokhano wa chipani cha DPP | Koma Meya wa mu mzindawu a Devi Maunde ati kunalibe Fukhanso miting’i koma unali msokhano wa chipani cha Dipipi | Female | |
Nduna ya Maboma ang'ono ndi Chitukuko chakumudzi a Richard Chimwendo Banda ati afufuze kaye kuti a Mayor ndi wachiwiri wawo anajomba chifukwa chani | Nduna ya Maboma ang'ono ndi Chitukuko chakumudzi a Litchadi Chimwendo Banda ati afufuze kaye kuti a Meya ndi wachiwiri wawo anajomba chifukwa chani | Female | |
Uladi Mussa yemwe anali mu Chipani Cha DPP walowa mchipani Cholamula Cha Malawi Congress Party (MCP) | Uladi Musa yemwe anali mu Chipani Cha Dipipi walowa mchipani Cholamula Cha Malawi kongilesi pate (emusipi) | Female | |
A Mussa alengeza lero ku Salima pamene mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera akuchititsa mtsonkhano wa chitukuko m'bomalo | A Musa alengeza lero ku Salima pamene mtsogoleri wa dziko lino Dokota Lazalasi Chakwera akuchititsa mtsonkhano wa chitukuko m'bomalo | Female | |
Mussa ndi mmodzi mwa anthu amene anaimisidwa ku chipani Chotsutsa Cha DPP. A Mussa omwe anadziwika kwa mbiri dzina loti chenji golo anakhalaso muchipani cha PP | Musa ndi mmodzi mwa anthu amene anaimisidwa ku chipani Chotsutsa Cha Dipipi. A Musa omwe anadziwika kwa mbiri dzina loti chenji golo anakhalaso muchipani cha Pipi | Female | |
Chipani cha Democratic Progressive (DPP) chachotsa a Kondwani Nankhumwa ndi anthu ena mu chipanichi ati chifukwa chosasunga mwambo | Chipani cha Demokilatiki pulogilesivi (Dipipi) chachotsa a Kondwani Nankhumwa ndi anthu ena mu chipanichi ati chifukwa chosasunga mwambo | Female | |
Wachiwiri kwa mtsogoleri wachipani cha UDF kuchigawo cha kum'mawa a Hasheem Banda watula pansi udindo wake komanso watuluka mchipanichi | Wachiwiri kwa mtsogoleri wachipani cha Yudiefu kuchigawo cha kum'mawa a Hashimu Banda watula pansi udindo wake komanso watuluka mchipanichi | Female | |
A Banda ayakhula izi lero pa msonkhano wa atolakhani ku Zomba. Iwo ati achita izi kamba koti anawakanazi kulowa ku msokhano wa Ukulu, National Executive Committee meeting | A Banda ayakhula izi lero pa msonkhano wa atolakhani ku Zomba. Iwo ati achita izi kamba koti anawakanazi kulowa ku msokhano wa Ukulu, Neshono ekizekitivi komiti miting’i | Female | |
omwe analetsedwa kuti asakhale nawo pa msonkhano umachitikira ku Blantyre pa 13 january 2023. Ndipo pa 18 september analembaso kalata yotuluka mchipanichi koma akulu akulu achipani | omwe analetsedwa kuti asakhale nawo pa msonkhano umachitikira ku Bulantaya pa fetini Januwale Twente twente fili Ndipo pa eitini sepitrmba analembaso kalata yotuluka mchipanichi koma akulu akulu achipani | Female | |
anawaitanisa nkukambirana nawo kuti asatuluke. A Banda ati panopa chipani china chili chonse chomwe chingawafikile agwira nawo ntchito limodzi | anawaitanisa nkukambirana nawo kuti asatuluke. A Banda ati panopa chipani china chili chonse chomwe chingawafikile agwira nawo ntchito limodzi | Female | |
Mneneri wachipani cha UDF a Yusuf Mwawa ati ngati iwo alengeza kuti atuluka mchipanichi ndi ufulu wawo ndipo akuwafunila za bwino zonse | Mneneri wachipani cha yudiefu a Yusufu Mwawa ati ngati iwo alengeza kuti atuluka mchipanichi ndi ufulu wawo ndipo akuwafunila za bwino zonse | Female | |
Mtsogoleri wakale wa mdziko lino Dr Joyce Banda wapeleka chimanga kwa mabanja opitilira 500 ku domasi kwa mfumu yayikulu Malemia m'boma la Zomba | Mtsogoleri wakale wa mdziko lino Dokota Joyisi Banda wapeleka chimanga kwa mabanja opitilira Faifi handiledi ku domasi kwa mfumu yayikulu Malemia m'boma la Zomba | Female | |
A Banda ati chimanga chomwe akugawa sichaboma koma ndichomwe amagula kudzera muthandizo losiyana siyana lomwe amapeza kudzera kwa anthu akufuna kwa bwino | A Banda ati chimanga chomwe akugawa sichaboma koma ndichomwe amagula kudzera muthandizo losiyana siyana lomwe amapeza kudzera kwa anthu akufuna kwa bwino | Female | |
Mtsogoleri otsutsa boma kunyumba yamalamulo, Dr Kondwani Nankhumwa asankha phungu wadera la Mangochi Monkey Bay a Ralph Jooma kukhala mneneri wawo | Mtsogoleri otsutsa boma kunyumba yamalamulo, Dokota Kondwani Nankhumwa asankha phungu wadera la Mangochi Monkibe a Rafu Joma kukhala mneneri wawo | Female | |
Izi ndi malingana ndi kalata kuchokera kwa mlembi othandizira Dr Nankhumwa, a Dorothy Kabango. Pali chiyembekezo choti masewero a Darts tsopano apita patsogolo | Izi ndi malingana ndi kalata kuchokera kwa mlembi othandizira Drokota Nankhumwa, a Dolofe Kabango. Pali chiyembekezo choti masewero a Datsi tsopano apita patsogolo | Female | |
potsatira chidwi cha anthu akufuna kwa bwino pa masewerowa mdziko muno. Izi zadziwika pomwe bank ya CDHIB yapereka cheque cha ndalama zokwana 5 Million kwacha | potsatira chidwi cha anthu akufuna kwa bwino pa masewerowa mdziko muno. Izi zadziwika pomwe banki ya sidietchiayibi yapereka cheke cha ndalama zokwana faifi miliyoni kwacha | Female | |
Ku bungwe la Darts Association of Malawi lachitatu lathali mu mzinda wa Blantyre. Polakhula pa mwambowu mmodzi mwa akuluakulu oyendetsa ntchito za malonda Ku bankiyi | Ku bungwe la Datsi Asosiyeshoni ofu Malawi lachitatu lathali mu mzinda wa Bulantaya. Polakhula pa mwambowu mmodzi mwa akuluakulu oyendetsa ntchito za malonda Ku bankiyi | Female | |
Nancy Bisika anati aganiza zobwera ndi thandizoli potengera kuti masewerowa ndi amodzi mwa masewero omwe akusowekera thandizo lalikulu ngati chilimbikitso cha ndalama Mwa zina chabe | Nanse Bisika anati aganiza zobwera ndi thandizoli potengera kuti masewerowa ndi amodzi mwa masewero omwe akusowekera thandizo lalikulu ngati chilimbikitso cha ndalama Mwa zina chabe | Female | |
Apa a Bisika anati ndichokhumba chawo chachikulu ngati bank kuti masewerowa apite patsogolo pofikira anthu ochuluka monga achinyamata ndi amayi kuti nawo azisewera masewerowa mdziko muno | Apa a Bisika anati ndichokhumba chawo chachikulu ngati banki kuti masewerowa apite patsogolo pofikira anthu ochuluka monga achinyamata ndi amayi kuti nawo azisewera masewerowa mdziko muno | Female | |
Polandira thandizoli, mlembi wamkulu Wa bungwe la Darts Association of Malawi Prestone Matande wayamikira bankiyi pobwetsa nthandizoli Ku nthawi yake | Polandira thandizoli, mlembi wamkulu Wa bungwe la Daatsi asosiyeshoni ofu Malawi Pulesitoni Matande wayamikira bankiyi pobwetsa nthandizoli Ku nthawi yake | Female | |
ponena kuti ndalamazi zithandizira pa mpikisano wa osewera osiyanasiyana omwe uyambike lachisanu pa 22 mwezi uno omwe mafainolo ake adzachitike sabata lomaliza la mwezi woyamba Wa chaka cha mmawa | ponena kuti ndalamazi zithandizira pa mpikisano wa osewera osiyanasiyana omwe uyambike lachisanu pa twente thu mwezi uno omwe mafainolo ake adzachitike sabata lomaliza la mwezi woyamba Wa chaka cha mmawa | Female | |
Bwalo la milandu la principal Residents Magistrate ku Zomba lero lalephera kupitilira kumva mulandu wa a Bon Kalindo omwe anamangidwa podzetsa ziwawa pa zionetsere zomwe anachitisa ku Zomba mwezi watha | Bwalo la milandu la princpulinsipo lezidenti majesitileti ku Zomba lero lalephera kupitilira kumva mulandu wa a Boni Kalindo omwe anamangidwa podzetsa ziwawa pa zionetsere zomwe anachitisa ku Zomba mwezi watha | Female | |
Omwe akuimira a Kalindo, a Timothy Chirwa anati bwaloli lakanika kupitilira kumva mlanduwu kamba koti oweruza mulandu a Martin Chipofya sakupeza bwino mthupi | Omwe akuimira a Kalindo, a Timofe Chirwa anati bwaloli lakanika kupitilira kumva mlanduwu kamba koti oweruza mulandu a Matini Chipofya sakupeza bwino mthupi | Female | |
Iwo anati adikira tsiku lomwe abwalo awauze tsiku lomwe mulanduwu uzapitilire. A Kalindo akuyembekezekanso kuti akayakhe mulandu onga ngati omwewo ku Mangochi pa 11 January | Iwo anati adikira tsiku lomwe abwalo awauze tsiku lomwe mulanduwu uzapitilire. A Kalindo akuyembekezekanso kuti akayakhe mulandu onga ngati omwewo ku Mangochi pa leveni januwale | Female | |
Chipani cha Democratic Progressive (DPP) chati chayimitsa msonkhano wake wapa 26 ndi pa 27 mwezi uno, omwe umati asankhe atsogoleri m'maudindo ena | Chipani cha Demokilatiki pulogilesivi (Dipipi) chati chayimitsa msonkhano wake wapa twente sikisi ndi pa twente seveni mwezi uno, omwe umati asankhe atsogoleri m'maudindo ena | Female | |
M'neneri wa chipani a Shadric Namalomba ati izi zikutsatira kuvomeleza kwa bwalo la milandu la High Court ku Lilongwe pempho loti awaonjezera masiku okonzekera msonkhano waukulu wosankha atsogoleri | M'neneri wa chipani a Shadileki Namalomba ati izi zikutsatira kuvomeleza kwa bwalo la milandu la Hayi khoti ku Lilongwe pempho loti awaonjezera masiku okonzekera msonkhano waukulu wosankha atsogoleri | Female | |
A Namalomba ati, atsogoleri mu komiti ya NGC akumana Chaka cha mawa kuti adzakhazikitse masiku atsopano | A Namalomba ati, atsogoleri mu komiti ya enijisi akumana Chaka cha mawa kuti adzakhazikitse masiku atsopano | Female | |
Fleetwood Haiya wasakhidwa ngati mtsogoleri watsopano wa bungwe la FAM atagwetsa a Walter Nyamilandi ndi mavoti 23 kwa 13 | Fulitiwudu Haiya wasakhidwa ngati mtsogoleri watsopano wa bungwe la FAMU atagwetsa a Wota Nyamilandi ndi mavoti twente fili kwa fetini | Female | |
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa bungweli ndi a Christopher Madalitso Kuyera atagonjetsa a James Mwenda ndi ma voti 19 kwa 17 | Wachiwiri kwa mtsogoleri wa bungweli ndi a Khilisitofa Madalitso Kuyera atagonjetsa a Jemusi Mwenda ndi ma voti naintini kwa seventini | Female | |
Wachiwiri kwa wachiwiri kwa mtsogoleri wa bungweli ndi Othaniel Hara ndi mavoti 21 kwa 15 | Wachiwiri kwa wachiwiri kwa mtsogoleri wa bungweli ndi Ofaniele Hara ndi mavoti twente wani kwa fifitini | Female | |
Ma membala a komiti ndi Daudu Mtantiko, Chimango Munthali, Benard chiwiliwili Harawa ndi Patrick Harawa. Ndipo a Felister Dosi ndi oimila azimayi Mubungwe la FAM | Ma membala a komiti ndi Daudu Mtantiko, Chimango Munthali, Benadi chiwiliwili Harawa ndi Patiliki Harawa. Ndipo a Felisita Dosi ndi oimila azimayi Mubungwe la FAMU | Female | |
Sukulu ya sekondale ya Mulunguzi ku Zomba yakhala masiku anayi tsopano opanda magetsi, zomwe zakhudza maphunziro pasukuluyi | Sukulu ya sekondale ya Mulunguzi ku Zomba yakhala masiku anayi tsopano opanda magetsi, zomwe zakhudza maphunziro pasukuluyi | Female | |
Mphunzitsi wamkulu pa sukuluyi a Silk Kadwala ati izi zikudza pamene sukuluyi isakulandira ndalama zogulira zofunikira kuchokera ku boma | Mphunzitsi wamkulu pa sukuluyi a Siuki Kadwala ati izi zikudza pamene sukuluyi isakulandira ndalama zogulira zofunikira kuchokera ku boma | Female | |
Kusowa kwa Chakudya komanso kuthima kwa magetsi kwasokoneza maphunziro. Pakadakali pano ana akuwalembetsa mayeso kuti pofika Lachisanu sabata ino ophunzirawa akhale atachoka pa sukulupo | Kusowa kwa Chakudya komanso kuthima kwa magetsi kwasokoneza maphunziro. Pakadakali pano ana akuwalembetsa mayeso kuti pofika Lachisanu sabata ino ophunzirawa akhale atachoka pa sukulupo | Female | |
Apolisi ku Zomba amanga bambo wazaka 35, Tamani Sulumba pomuganizira kuti amafuna kulowesa ma simu kadi alamya za m'manja okwana 99 mwachinyengo ku ndende ya Zomba | Apolisi ku Zomba amanga bambo wazaka fete faifi, Tamani Sulumba pomuganizira kuti amafuna kulowesa ma simu kadi alamya za m'manja okwana nainte naini mwachinyengo ku ndende ya Zomba | Female | |
M'meneri wa Polisi ku Zomba Sub-Inspector Patricia Sipiliano, watsimikiza zakumangidwa kwa bamboyi | M'meneri wa Polisi ku Zomba Sabu insipekita Patilisha Sipiliyano, watsimikiza zakumangidwa kwa bamboyi | Female | |
iwo ati, woganizilidwayu anagwidwa ndi asilikali andende pomwe anabwera kuzaona mzake yemwe akumusunga pa ndendeyi | iwo ati, woganizilidwayu anagwidwa ndi asilikali andende pomwe anabwera kuzaona mzake yemwe akumusunga pa ndendeyi | Female | |
ndipo anatenga botolo la mafuta a mtundu wa Skala Body Cream ngati mphatso momwe anabisamo ma simu kadi | ndipo anatenga botolo la mafuta a mtundu wa Sikala Bode kilimu ngati mphatso momwe anabisamo ma simu kadi | Female | |
Sipiliano wati pakadali pano woganizilidwayu akaonekera ku bwalo la mlandu posachedwapa. Sulumba amachokera m'mudzi wa Masanjala, mfumu yaikulu Mpama m'boma la Chiradzulu | Sipiliyano wati pakadali pano woganizilidwayu akaonekera ku bwalo la mlandu posachedwapa. Sulumba amachokera m'mudzi wa Masanjala, mfumu yaikulu Mpama m'boma la Chiradzulu | Female | |
Mtsogoleri wa Chipani Cha Democratic Progressive Party (DPP) Professor Peter Muthalika achosa a Kondwani Nankhumwa ngati wachiwiri kwa Mtsogoleri wachipani ku Chigawo cha kumwera | Mtsogoleri wa Chipani Cha Demokilatiki pulogilesivi pate (Dipipi) Pulofesa pita Muthalika achosa a Kondwani Nankhumwa ngati wachiwiri kwa Mtsogoleri wachipani ku Chigawo cha kumwera | Female | |
Malingana ndi Kalata yomwe ufulu online yaona yasainidwa ndi a Muthalika. A George Chaponda alowa m'malo mwa a Nankhumwa | Malingana ndi Kalata yomwe ufulu onilayini yaona yasainidwa ndi a Muthalika. A Joji Chaponda alowa m'malo mwa a Nankhumwa | Female | |
ngati mtsogoleri wachiwiri ku Chigawo cha kumwera. Ndipo a Nankhumwa ndi mulangizi wa a Muthalika.Komanso a Cecilia Chazama ndi mulangizi wa a Munthalika | ngati mtsogoleri wachiwiri ku Chigawo cha kumwera. Ndipo a Nankhumwa ndi mulangizi wa a Muthalika.Komanso a sisiliya Chazama ndi mulangizi wa a Munthalika | Female | |
Mtsogoleri wakale wa dziko lino Dr. Joyce Banda apeleka chimanga kwa mawanja opitilira zikwi ziwiri, 2 thousand Ku Domasi kwa mfumu yayikulu malemia m'boma la Zomba | Mtsogoleri wakale wa dziko lino Dokota Joyisi Banda apeleka chimanga kwa mawanja opitilira zikwi ziwiri, Thu sauzande Ku Domasi kwa mfumu yayikulu malemia m'boma la Zomba | Female | |
Poyakhula kwa anthu omwe anafika ku nyumba kwao. A Banda ati boma likuthandiza anthu ovutika ndi njala koma ndipofunika anthu ena omwe ali ndi kuthekera azitengapo gawo lothandizaso | Poyakhula kwa anthu omwe anafika ku nyumba kwao. A Banda ati boma likuthandiza anthu ovutika ndi njala koma ndipofunika anthu ena omwe ali ndi kuthekera azitengapo gawo lothandizaso | Female | |
Bwalo la Principal Resident Magistrate ku Zomba lapeleka belo kwa Bon Kalindo. Principal Resident Magistrate Martin Chipofya | Bwalo la Pulinsipo lesidenti majesitilet ku Zomba lapeleka belo kwa Boni Kalindo. Pulinsipo lesidenti majesitilet Matini Chipofya | Female | |
wapeleka belo pa mulandu omwe amawazenga owaganizila kuti a Kalindo anayambisa ziwawa kutsatira zionesero zomwe zidachitika mu mzinda wa Zomba | wapeleka belo pa mulandu omwe amawazenga owaganizila kuti a Kalindo anayambisa ziwawa kutsatira zionesero zomwe zidachitika mu mzinda wa Zomba | Female | |
A Kalindo awauza kuti apeleke Chikole cha ndalama zokwana k400,000 ndipo azikaonekeranso ku Polisi ku Chigawo cha ku mvuma, Lachisano sabata ziwiri | A Kalindo awauza kuti apeleke Chikole cha ndalama zokwana folo handiledi sauzande kwacha ndipo azikaonekeranso ku Polisi ku Chigawo cha ku mvuma, Lachisano sabata ziwiri | Female | |
Oweruza mlanduwu akuti a Kalindo abweretse m'bale wawo ngati mboni imene ipeleke k1 million. Padakali pano a Polisi awamanga a Kalindo akupita nawo ku mangochi | Oweruza mlanduwu akuti a Kalindo abweretse m'bale wawo ngati mboni imene ipeleke wani miliyoni kwacha. Padakali pano a Polisi awamanga a Kalindo akupita nawo ku mangochi | Female | |
Mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive Party - DPP Proffesor Peter Mutharika achotsa pampando mlembi wamkulu wachipanichi a Grezelder Jeffrey ndipo m'malo mwake wayikapo Dr Clement Mwale | Mtsogoleri wa chipani cha Demokilatiki pulogilesivi pate -Dipipi Pulofesa Pita Mutharika achotsa pampando mlembi wamkulu wachipanichi a Gilezeda Jefule ndipo m'malo mwake wayikapo Dokota Kilementi Mwale | Female | |
A Jeffrey, tsopano ndi wa wachiwiri kwa mtsogoleri wachipanichi chigawo chapakati. Malingana ndi m'neneri wa a Mutharika a Shadric Namalomba, a Mutharika achita izi malingana ndi mphamvu zomwe alinazo | A Jefule, tsopano ndi wa wachiwiri kwa mtsogoleri wachipanichi chigawo chapakati. Malingana ndi m'neneri wa a Mutharika a Shadileki Namalomba, a Mutharika achita izi malingana ndi mphamvu zomwe alinazo | Female | |
Bungwe la Fedoma lati lili ndi chiyembekezo chachikulu patsolo la anthu omwe ali ndi ulumali osiyanasiyana pomwe bilu yatsopano yavomeredwa | Bungwe la Fedoma lati lili ndi chiyembekezo chachikulu patsolo la anthu omwe ali ndi ulumali osiyanasiyana pomwe bilu yatsopano yavomeredwa | Female | |
kukhala lamulo ndicholinga chikonzanso zovuta zomwe anthuwa amakumana nazo pa moyo wawo wa tsiku ndi tsiku Mmodzi Mwa akulukulu Ku bungwe loona za chisamalirochi la FEDOMA | kukhala lamulo ndicholinga chikonzanso zovuta zomwe anthuwa amakumana nazo pa moyo wawo wa tsiku ndi tsiku Mmodzi Mwa akulukulu Ku bungwe loona za chisamalirochi la FEDOMA | Female | |
Lyson Mapanga ndiye watsimikiza izi pomwe amafotoza zambiri za tsiku la pa 8 December lomwe dziko lino likhale likukumbukira za umoyo wa anthuwa mboma la Mulanje | Laisoni Mapanga ndiye watsimikiza izi pomwe amafotoza zambiri za tsiku la pa eiti Disemba lomwe dziko lino likhale likukumbukira za umoyo wa anthuwa mboma la Mulanje | Female | |
Amapanga ati mu bilu ya kale munali zosamwitsa zina monga kuchuluka kwa ntchito zomwe zimaonedwa ndi unduna umodzi womwe ndi woona za kusasiyana pakati pa a mayi ndi abambo | Amapanga ati mu bilu ya kale munali zosamwitsa zina monga kuchuluka kwa ntchito zomwe zimaonedwa ndi unduna umodzi womwe ndi woona za kusasiyana pakati pa a mayi ndi abambo | Female | |
komanso chisamaliro cha anthu zomwe ati zikuyenera kugawidwa tsopano lamuloli likayamba kugwira ntchito mwa zina | komanso chisamaliro cha anthu zomwe ati zikuyenera kugawidwa tsopano lamuloli likayamba kugwira ntchito mwa zina | Female | |
Bungwe la United Nations kudzera mu gwirizano wa maiko linakhazikitsa 3 December mchaka cha 1992 ngati tsiku lounikira za umoyo wa anthu | Bungwe la Yunaitedi neshonzi kudzera mu gwirizano wa maiko linakhazikitsa fili Disemba mchaka cha naintini nainte thu ngati tsiku lounikira za umoyo wa anthu | Female | |
omwe ali ndi ulumali wosiyanasiyana ndipo boma la Malawi mchaka cha 2015 lanakhazikitsanso masiku a pa 3 November mpaka 3 December | omwe ali ndi ulumali wosiyanasiyana ndipo boma la Malawi mchaka cha twente fifitini lanakhazikitsanso masiku a pa 3fili novemba mpaka fili disemba | Female | |
kukhala mwezi wokombukira zambiri za anthuwa mwapadera. Nthambi ya Malawi Police Services M'dziko muno yasamusa ogwira ntchito atatu | kukhala mwezi wokombukira zambiri za anthuwa mwapadera. Nthambi ya Malawi Polisi Sevisi M'dziko muno yasamusa ogwira ntchito atatu | Female | |
kuchokera ku police ya Chigawo cha ku m'mawa kupita ku ma boma ena M'dziko muno. Mwa ena omwe asamusidwa ku Chigawo Chaku mmawa, Eastern Regional Commissioner of Police | kuchokera ku polisi ya Chigawo cha ku m'mawa kupita ku ma boma ena M'dziko muno. Mwa ena omwe asamusidwa ku Chigawo Chaku mmawa, Isiteni lijono komishona ofu polisi | Female | |
Vailet Magwaya akupita ku Area 30, wachiwiri wake Kelvin Mulezo akupita ku Karonga ndinso mkulu wa police Mobile Othana ndi Chisawawa wa Chigawo cha ku m'mawa | Vaileti Magwaya akupita ku eliya fete, wachiwiri wake Keovini Mulezo akupita ku Karonga ndinso mkulu wa polisi Mobailo Othana ndi Chisawawa wa Chigawo cha ku m'mawa | Female | |
Senior Supritendant Benson Makawa.a kupita ku mchinji. Mneneri wa mkulu wa nthambi ya Malawi Police Services M'dziko muno | Siniyo supulitendanti Benisoni Makawa. akupita ku mchinji. Mneneri wa mkulu wa nthambi ya Malawi Polisi sevisi M'dziko muno | Female | |
A Peter Kalaya atsimikiza za kusamusidwa kwa apolisiwa. Koma akana kuthilira ndemanga. Masabata apitawa apolisi anathira utsi okhetsa misonzi boma la Zomba ndi Mangochi | A Peita Kalaya atsimikiza za kusamusidwa kwa apolisiwa. Koma akana kuthilira ndemanga. Masabata apitawa apolisi anathira utsi okhetsa misonzi boma la Zomba ndi Mangochi | Female | |
Kutsatira zionetsero zomwe zinachitika zomwe adakonza ndi Bon Kalindo. Bungwe la Malawi National Council of Sports (MNCS) | Kutsatira zionetsero zomwe zinachitika zomwe adakonza ndi Boni Kalindo. Bungwe la Malawi Nationeshono khanso ofu sipotsi (Emueni siesi) | Female | |
lauza wapa mpando wa Southern Region Football Association (SRFA) Raphael Humba kuti afotokoze njira zomwe anagwiritsa ntchito posankha a Walter Nyamilandu | lauza wapa mpando wa Sauveni lijono futubo asosiyeshoni (Esi alaefue) Lafaelo Humba kuti afotokoze njira zomwe anagwiritsa ntchito posankha a Wota Nyamilandu | Female | |
kuti adzapikitsane nawo pa chisankho chomwe Football Association of Malawi (FAM) lichitise pa 16 December 2023 mu mzinda wa Mzuzu | kuti adzapikitsane nawo pa chisankho chomwe Futubo asosiyeshoni ofu Malawi (FAMU) lichitise pa sikisitini Disemba twente twente fili mu mzinda wa Mzuzu | Female | |
Malingana ndi MNCS kalata atulutsa yomwe bungwe lothana katangale ndi ziphuphu dziko muno la Anti Corruption Bureau (ACB) ladandaulira kubungweli | Malingana ndi emueni siesi kalata atulutsa yomwe bungwe lothana katangale ndi ziphuphu dziko muno la Anti Kopushoni Byulo (Esibi) ladandaulira kubungweli | Female | |
ACB yatula madando kubungwe la MNCS yoti yalandira dandaulo lomwe likufotokoza kuti a Humba akhala akugwiritsa ntchito mpando wawo molakwika | Esibi yatula madando kubungwe la Emueni siesi yoti yalandira dandaulo lomwe likufotokoza kuti a Humba akhala akugwiritsa ntchito mpando wawo molakwika | Female | |
ponyozera ena mwa malamulo a SRFA pokondera a Nyamilandu pa chisankho chomwe FAM ikhale nacho pansonkhano wake waukulu omwe uchitike mwezi wa December ku Mzuzu | ponyozera ena mwa malamulo a Esiala efue pokondera a Nyamilandu pa chisankho chomwe FAMU ikhale nacho pansonkhano wake waukulu omwe uchitike mwezi wa Disemba ku Mzuzu | Female | |
Chikalatachi chikufotozanso kuti chaka cha chisankho ku FAM, a Humba amanyozera malamulo mwadala posankha nthumwi zomwe amadziwa kuti zikapereka voti yawo | Chikalatachi chikufotozanso kuti chaka cha chisankho ku FAMU, a Humba amanyozera malamulo mwadala posankha nthumwi zomwe amadziwa kuti zikapereka voti yawo | Female | |
kwa a Nyamilandu kusiyana kutenga oyenera. MNCS yapempha a Humba kuti apereke ndondomeko ya m'mene anachitira zinthu zawo | kwa a Nyamilandu kusiyana kutenga oyenera. Emueni siesi yapempha a Humba kuti apereke ndondomeko ya m'mene anachitira zinthu zawo | Female | |
kuphatikizirapo pomwe amalemba patsiku lomwe amakambilana zosankha a Nyamilandu kuti akapikisane nawo pa chisankhochi | kuphatikizirapo pomwe amalemba patsiku lomwe amakambilana zosankha a Nyamilandu kuti akapikisane nawo pa chisankhochi | Female | |
Bungweli lapephanso SRFA kuti itumize ndondomeko ya malamulo awo ndicholinga choti akaone ngati zomwe zinachitika patsikuli zili m'malamulo oyendesera bungweli | Bungweli lapephanso esiala efue kuti itumize ndondomeko ya malamulo awo ndicholinga choti akaone ngati zomwe zinachitika patsikuli zili m'malamulo oyendesera bungweli | Female | |
MNCS yauza SRFA kuti zikalatazi zitumizidwe kubungweli pasanadutse lachisanu pa 1 December 2023 | Emueni siesi yauza esiala efue kuti zikalatazi zitumizidwe kubungweli pasanadutse lachisanu pa wani Disemba Twente twente fili | Female | |
Bungwe lomwe likuyendetsa chisankho cha mtsogoleri wa bungwe loyendetsa masewero mdziko muno (FAM) lakana pepho la Walter Nyamilandu Manda | Bungwe lomwe likuyendetsa chisankho cha mtsogoleri wa bungwe loyendetsa masewero mdziko muno (FAMU) lakana pepho la Wota Nyamilandu Manda | Female | |
lopempha bungweli kuti livomereze Fleetwood Haiya kupikisana nao pa mpando waukulu ku bungweli | lopempha bungweli kuti livomereze Fulitihudu Haiya kupikisana nao pa mpando waukulu ku bungweli | Female | |
Malingana ndi chikalata chomwe a Nyamilandu analembera bungwe lomwe likuyendetsa chisankho Makiyi Kanyenda and Associates cha FAM | Malingana ndi chikalata chomwe a Nyamilandu analembera bungwe lomwe likuyendetsa chisankho Makiyi Kanyenda and asosiyetsi cha FAMU | Female | |
ku dzera mwa a owaimilira pankhani za Malamulo chinati mwamfundo zina a Haiya sakuyenera kukapikisana nao pa mpando waukulu ku bungweli | ku dzera mwa a owaimilira pankhani za Malamulo chinati mwamfundo zina a Haiya sakuyenera kukapikisana nao pa mpando waukulu ku bungweli | Female | |
kamba koti adakali mtsogoleri wa team ya FCB Nyasa Big Bullets komanso mkulu wa bungwe loyendetsa masewero a league yaikulu mdziko muno Super League | kamba koti adakali mtsogoleri wa team ya Efusibi Nyasa Bigi Buletsi komanso mkulu wa bungwe loyendetsa masewero a league yaikulu mdziko muno Supaligi | Female | |
bungwe lapadera lomwe likuyendetsa zisankhozi lati mfundo zomwe apereka a Nyamilandu ndi zosamveka | bungwe lapadera lomwe likuyendetsa zisankhozi lati mfundo zomwe apereka a Nyamilandu ndi zosamveka | Female | |
Ngati njira imodzi yofuna kutengapo gawo pobwezeretsa chilengedwe m'dziko muno, bungwe la Hope Ministries International lachititsa maphunziro kwa aphunzitsi a msukulu za pulaimale | Ngati njira imodzi yofuna kutengapo gawo pobwezeretsa chilengedwe m'dziko muno, bungwe la Hopu Minisitilezi intaneshono lachititsa maphunziro kwa aphunzitsi a msukulu za pulaimale | Female | |
ndondomeko yobzala mitengo ndi mbewu. M'modzi mwa akulu akulu a Board ya Hope Ministries International a Blessings Mlowoka wati cholinga chamaphunzirowa ndikupeleka ukadaulo obzala mitengo | ndondomeko yobzala mitengo ndi mbewu. M'modzi mwa akulu akulu a Bodi ya Hopu Minisitilezi intaneshono a Bulesing’izi Mlowoka wati cholinga chamaphunzirowa ndikupeleka ukadaulo obzala mitengo | Female | |
ndikulimila mbewu limodzi kwa aphunzitsi kuti akaphunzitse ana m'sukulu zawo. Iye wati m'sukulu zambiri zikhala nawo mndondomeko yophunzira kudzala mitengo ndinso ubwino osamalira za Chilengedwe | ndikulimila mbewu limodzi kwa aphunzitsi kuti akaphunzitse ana m'sukulu zawo. Iye wati m'sukulu zambiri zikhala nawo mndondomeko yophunzira kudzala mitengo ndinso ubwino osamalira za Chilengedwe | Female | |
Maphunzirowa akuwatcha kuti Agro-Forestry kulimira limodzi mbewu komanso nkhalango ndikuteteza nthaka kuti ikhale yolimba kuti mavuto omwe akumagwa mwadzi dzidzi azitha kuwaphelera | Maphunzirowa akuwatcha kuti Agulo folesitile kulimira limodzi mbewu komanso nkhalango ndikuteteza nthaka kuti ikhale yolimba kuti mavuto omwe akumagwa mwadzi dzidzi azitha kuwaphelera | Female | |
Ndipo mayi Christina Kamwendo yemwe ndi mlangizi wa za maphunziro ku Namadidi Zone boma la Zomba, wati maphunzirowa athandiza kwambiri kwa ana | Ndipo mayi Khilisitina Kamwendo yemwe ndi mlangizi wa za maphunziro ku Namadidi Zoni boma la Zomba, wati maphunzirowa athandiza kwambiri kwa ana | Female | |
maka omwe ataphunzire ulimi olimbikitsa kusamala mitengo ndi mbewu ku sukulu ndi kumadera. Pali chiyembekezo choti imfa za ana omwe ndi osaposera zaka 14 tsopano zichepa | maka omwe ataphunzire ulimi olimbikitsa kusamala mitengo ndi mbewu ku sukulu ndi kumadera. Pali chiyembekezo choti imfa za ana omwe ndi osaposera zaka fotini tsopano zichepa | Female | |
watero mkulu wa Chipatala chachikulu cha queens mu mzinda wa Blantyre,Dr Kelvin Mponda. Mponda watsimikiza izi lachisanu mu mzindawu | watero mkulu wa Chipatala chachikulu cha Kwinzi mu mzinda wa Bulantaya, Dokota Keovini Mponda. Mponda watsimikiza izi lachisanu mu mzindawu | Female | |
pamwambo otsegulira nyumba yotsopano yothandizira anawa akadwala mwadzidzidzi kapena kuvulala pangozi zosiyanasiyana ,yomwe yamagwidwa ndi ndalama pafufupi 1 Billion kwacha ndi mabanja ena akufuna kwabwino | pamwambo otsegulira nyumba yotsopano yothandizira anawa akadwala mwadzidzidzi kapena kuvulala pangozi zosiyanasiyana ,yomwe yamagwidwa ndi ndalama pafufupi wani Biliyoni kwacha ndi mabanja ena akufuna kwabwino | Female | |
Dr Mponda anati ana pafupifupi ana 50 pa 100 aliwonse akhala akumwalira pa maola 24 oyamba patsiku lomwe atengeredwa kuchipatachi podikirira kulandira thandizo la chipatala | Dokota Mponda anati ana pafupifupi ana fifite pa wani handiledi aliwonse akhala akumwalira pa maola twente folo oyamba patsiku lomwe atengeredwa kuchipatachi podikirira kulandira thandizo la chipatala | Female | |
choncho kubwera kwa chipatalachi kuchepesa vutoli kaamba koti pachipatalichi panali malo antundu amodzi okha | choncho kubwera kwa chipatalachi kuchepesa vutoli kaamba koti pachipatalichi panali malo antundu amodzi okha | Female | |
Ndipo mmawa ake yemwe anali mlendo wolemekeza nduna ya za umoyo Mai Khumbidze Kandodo anayamikira mabanjawa kaamba Ka thandizoli | Ndipo mmawa ake yemwe anali mlendo wolemekeza nduna ya za umoyo Mai Khumbidze Kandodo anayamikira mabanjawa kaamba Ka thandizoli | Female | |
komanso apempha mabungwe ndi anthu ena akufuna kwabwino kuti atengeropo chitsanzo. Chipatalachi chimalandira ana oposa 1000 omwe akhala akhukhudzidwa ndi Matenda adzidzidzi komanso ngozi | komanso apempha mabungwe ndi anthu ena akufuna kwabwino kuti atengeropo chitsanzo. Chipatalachi chimalandira ana oposa wani sauzande omwe akhala akhukhudzidwa ndi Matenda adzidzidzi komanso ngozi | Female | |
Nkhonsolo ya mzinda wa Blantyre yatsutsa mphekesera zoti ogwira ntchito ake omwe ndi azachitetezo cha anthu ochita malonda amwalira pa kusamvana komwe kunachitika la chitatu lapitali ku Limbe | Nkhonsolo ya mzinda wa Bulantaya yatsutsa mphekesera zoti ogwira ntchito ake omwe ndi azachitetezo cha anthu ochita malonda amwalira pa kusamvana komwe kunachitika la chitatu lapitali ku Limbi | Female | |
Izi zikudza pomwe a malonda ena mu mzindawu anagenda galimoto ya azachitetezowa ndikuwavulaza pomwe amachotsa anthu ena omwe amagulitsa malonda awo mmalo osayenera | Izi zikudza pomwe a malonda ena mu mzindawu anagenda galimoto ya azachitetezowa ndikuwavulaza pomwe amachotsa anthu ena omwe amagulitsa malonda awo mmalo osayenera | Female | |
Mkulu wa mzindawu Dennis Chinseu watsimikiza izi polankhula ndi Ufulu online, pomwe amapereka tsatanetsatane wa chitsogolo cha kukonzanso ubale wa mavenda ndi ogwira ntchitowa | Mkulu wa mzindawu Denisi Chinseu watsimikiza izi polankhula ndi Ufulu onilayini, pomwe amapereka tsatanetsatane wa chitsogolo cha kukonzanso ubale wa mavenda ndi ogwira ntchitowa | Female | |
pomwe wati akukonza ganizo lokhala ndi malo okhazikika oti anthuwa azikachitirako malonda awo ndipo ayamba kale kuchita zokambirana ndi mavendawa | pomwe wati akukonza ganizo lokhala ndi malo okhazikika oti anthuwa azikachitirako malonda awo ndipo ayamba kale kuchita zokambirana ndi mavendawa | Female | |
Ndipo mmawu ake,Sergeant Aubrey Singanyama yemwe ndi ofalitsa nkhani za apolisi Ku Limbe watsimikizira ufulu online | Ndipo mmawu ake,Sajenti Obule Singanyama yemwe ndi ofalitsa nkhani za apolisi Ku Limbi watsimikizira ufulu onilayini | Female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.