audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
kupatula kuwonjezera chiwelengero cha azachitetezo ku nkhalangoyi. A Postan Jere, m’modzi mwa mamembala amaanja omwe anakhudzidwa pamikanganoyi, ati akukumana ndi mavuto azachuma
kupatula kuwonjezera chiwelengero cha azachitetezo ku nkhalangoyi. A Positani Jere, m’modzi mwa mamembala amaanja omwe anakhudzidwa pamikanganoyi, ati akukumana ndi mavuto azachuma
Female
ndipo wapempha boma kuti iike pa mtima miyoyo yawo osati yanyamazi. Kuchokera pomwe boma linasamutsira munkhalango ya Kasungu njovu zoposa 250
ndipo wapempha boma kuti iike pa mtima miyoyo yawo osati yanyamazi. Kuchokera pomwe boma linasamutsira munkhalango ya Kasungu njovu zoposa thu handede andi fifite
Female
kuchoka ku nkhalango ya Liwonde mu chaka cha 2021, anthu okwana asanu ndi m’modzi, 6 anaphedwa komanso katundu ochuluka kuphatikizapo mbewu zinawonongedwa
kuchoka ku nkhalango ya Liwonde mu chaka cha twente twente wani, anthu okwana asanu ndi m’modzi sikisi anaphedwa komanso katundu ochuluka kuphatikizapo mbewu zinawonongedwa
Female
Ophunzira pafupifupi 1, 814 a msukulu za ukachenjede za boma komaso zomwe si za boma
Ophunzira pafupifupi wani sauzande eiti handede andi fotini a msukulu za ukachenjede za boma komaso zomwe si za boma
Female
asiidwa pa mndandanda wa ophunzira omwe apindule nawo ndi ngongole yomwe bungwe lopeleka ngongole kwa ophunzira la Higher Education Students Loans and Grants Board
asiidwa pa mndandanda wa ophunzira omwe apindule nawo ndi ngongole yomwe bungwe lopeleka ngongole kwa ophunzira la Haya ejukeshoni situdentsi lonzi andi gilantsi bodi
Female
lipeleke m’chaka cha maphunziro cha 2023 mpaka 2024, kaamba kosafikila mulingo oyenelera. Pomwe amalengeza izi Lachiwiri ku Mangochi
lipeleke m’chaka cha maphunziro cha twente twente fili mpaka twente twente folo, kaamba kosafikila mulingo oyenelera. Pomwe amalengeza izi Lachiwiri ku Mangochi
Female
wapampando komanso m’neneri wa komiti yopeleka ngongole ku bungweli, Dr. Henry Chingaipe wati mwa ophunzira 27, 075 omwe analembera ngongoleyi
wapampando komanso m’neneri wa komiti yopeleka ngongole ku bungweli, Dokota Henele Chingaipe wati mwa ophunzira twente seveni sauzande andi sevente faifi omwe analembera ngongoleyi
Female
25, 265 ndi omwe avomelezedwa zomwe zikuimira 93.3 pelesenti. Koma mtsogoleri wa nthambi ya ophunzira pa sukulu ya Malawi University of Business and Applied Sciences MUBAS
Twente faifi sauzande thu handed andi sikisite faifi ndi omwe avomelezedwa zomwe zikuimira nainte fili pointi fili pelesenti. Koma mtsogoleri wa nthambi ya ophunzira pa sukulu ya Malawi yunivesite ofu bizinezi andi apulayidi sayansezi, MUBASI
Female
Wyson Vinthenga wati ndi osakhutira ndi ndondomeko yomwe imagwiritsidwa ntchito posankha ophunzirawa. Iye wati ndale ndi zomwe zimagwira ntchito
Wayisoni Vinthenga wati ndi osakhutira ndi ndondomeko yomwe imagwiritsidwa ntchito posankha ophunzirawa. Iye wati ndale ndi zomwe zimagwira ntchito
Female
kaamba koti ena mwa ophunzira omwe amasankhidwa amakhala ana a anthu odziwika bwino pa ndale komanso chuma. Vinthenga akufuna kuti bungwe lopeleka ngongoleyi
kaamba koti ena mwa ophunzira omwe amasankhidwa amakhala ana a anthu odziwika bwino pa ndale komanso chuma. Vinthenga akufuna kuti bungwe lopeleka ngongoleyi
Female
lizigwiritsa ntchito akuluakulu a msukulu za ukachenjede komanso nthambi za ophunzira a msukuluzi posankha ophunzirawa, powonjezera kuti ena mwa ophunzira omwe asiidwa chaka chino amayenera kupindula nawo
lizigwiritsa ntchito akuluakulu a msukulu za ukachenjede komanso nthambi za ophunzira a msukuluzi posankha ophunzirawa, powonjezera kuti ena mwa ophunzira omwe asiidwa chaka chino amayenera kupindula nawo
Female
Chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive DPP chapempha Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus Chakwera kuti achotse pa udindo mkulu wa a polisi mdziko muno
Chipani chotsutsa boma cha Demokilatiki pulogilesivi Dipipi chapempha Mtsogoleri wa dziko lino Dokota Lazalasi Chakwera kuti achotse pa udindo mkulu wa a polisi mdziko muno
Female
mayi Merlyn Yolamu komaso nduna ya za chitetezo cha mdziko Dr. Ken Zikhale Ng’oma. Mu m’chikalata chomwe chipanichi chatulutsa masana a lachisanu
mayi Merini Yolamu komaso nduna ya za chitetezo cha mdziko Dokota Keni Zikhale Ng’oma. Mu m’chikalata chomwe chipanichi chatulutsa masana a lachisanu
Female
ndipo chasainilidwa ndi mneneri wake Shadreck Namalomba, Chipani chi chati mwa zina, ndichodabwa ndizomwe a police dzulo, lachinayi anachita pomwe gulu lotchedwa Malawi First
ndipo chasainilidwa ndi mneneri wake Shadileki Namalomba, Chipani chi chati mwa zina, ndichodabwa ndizomwe a polisi dzulo, lachinayi anachita pomwe gulu lotchedwa Malawi Fesiti
Female
linakonza ziwonetsero zofuna kuti Dr Chakwera atule pansi udindo wake, pomwe a police wa m’malo moteteza gululi amangowonerera anthu ena omwe chikhulupilira kuti anachita kutumidwa ndi Mkulu wa apolice
linakonza ziwonetsero zofuna kuti Dokota Chakwera atule pansi udindo wake, pomwe a polisi wa m’malo moteteza gululi amangowonerera anthu ena omwe chikhulupilira kuti anachita kutumidwa ndi Mkulu wa apolisi
Female
komanso Nduna ya Zachititezo cha dziko- wa anayamba kuvunga miyala kwa gulu lochita zionetserori. Koma pakadali pano, Nduna ya zofalitsa nkhani yemweso ndi mneneri wa boma, Moses Kumkuyu
komanso Nduna ya Zachititezo cha dziko- wa anayamba kuvunga miyala kwa gulu lochita zionetserori. Koma pakadali pano, Nduna ya zofalitsa nkhani yemweso ndi mneneri wa boma, Mozesi Kumkuyu
Female
wati sanalandire komanso kuiwona kalatayi. Lachinayi gulu lomenyera ufulu wa anthu la Malawi First motsogozedwa ndi Bon Kalindo linakoza zionetsero mu mzinda wa Lilongwe zomwe zinathera mpungwepungwe
wati sanalandire komanso kuiwona kalatayi. Lachinayi gulu lomenyera ufulu wa anthu la Malawi Fesiti motsogozedwa ndi Boni Kalindo linakoza zionetsero mu mzinda wa Lilongwe zomwe zinathera mpungwepungwe
Female
Anthu okhala m’boma la Kasungu adzudzula bungwe logawa madzi la mchigawo chapakati la Central Region Water Board ponena kuti likuwapatsa madzi osatetezeka pa miyoyo yawo
Anthu okhala m’boma la Kasungu adzudzula bungwe logawa madzi la mchigawo chapakati la Sentilo lijoni wota bodi ponena kuti likuwapatsa madzi osatetezeka pa miyoyo yawo
Female
M’modzi mwa amayi okhudzidwa m’bomali yemwe anapempha kuti tisamutchule dzina, wati madzi omwe anthuwa akumatunga m'mipopi akumakhala osakanikirana ndi mphutsi zowoneka zofiira
M’modzi mwa amayi okhudzidwa m’bomali yemwe anapempha kuti tisamutchule dzina, wati madzi omwe anthuwa akumatunga m'mipopi akumakhala osakanikirana ndi mphutsi zowoneka zofiira
Female
zinthu zomwe wati zikuika pachiopyezo thanzi lawo. Pakadali pano, Mneneri wa bungwe logawa madzi mchigawo chapakati, Zepherino Mitumba wati sadalandilepo dandaulo lililonse pankhaniyi
zinthu zomwe wati zikuika pachiopyezo thanzi lawo. Pakadali pano, Mneneri wa bungwe logawa madzi mchigawo chapakati, Zeferino Mitumba wati sadalandilepo dandaulo lililonse pankhaniyi
Female
Midzi ina m'boma la Nkhotakota ikusimba lokoma, anthu a m'midziyi atakwanitsa kukhazikitsa ntchito za chitukuko cha ku mtima kwawo
Midzi ina m'boma la Nkhotakota ikusimba lokoma, anthu a m'midziyi atakwanitsa kukhazikitsa ntchito za chitukuko cha ku mtima kwawo
Female
mothandizidwa ndi bungwe la Foundation for Community and Capacity Development, FOCCAD. Midziyi ndi ya Simba, Bamba 2, Bweya, komanso Nyemba kungotchulapo yochepa chabe
mothandizidwa ndi bungwe la Faundeshoni fo komyunite andi kapasite divelopumenti, FOKADI. Midziyi ndi ya Simba, Bamba 2, Bweya, komanso Nyemba kungotchulapo yochepa chabe
Female
yomwe ili pansi pa mfumu Malengachanzi ndi Mwadzama. Mwa chitsanzo, titayendera midziyi lero komwe kukugwilidwa ntchito monga ulimi wa mbuzi, Ng'ombe za mkaka komanso Nkhuku zamazila
yomwe ili pansi pa mfumu Malengachanzi ndi Mwadzama. Mwa chitsanzo, titayendera midziyi lero komwe kukugwilidwa ntchito monga ulimi wa mbuzi, Ng'ombe za mkaka komanso Nkhuku zamazila
Female
tapeza kuti anthu m'maderawa, ayamba kale kugulitsa mazila mwa zina, ndipo ndalama zake akuthandizira maanja awo. A mfumu a Simba 3 ati, zaka zitatu zikudzadzi
tapeza kuti anthu m'maderawa, ayamba kale kugulitsa mazila mwa zina, ndipo ndalama zake akuthandizira maanja awo. A mfumu a Simba fili ati, zaka zitatu zikudzadzi
Female
anthu m'derali sadzakhalanso chimodzimodzi pa nkhani zachuma, kaamba ka ulimi wa nkhuku za mazila omwe akuchita
anthu m'derali sadzakhalanso chimodzimodzi pa nkhani zachuma, kaamba ka ulimi wa nkhuku za mazila omwe akuchita
Female
Mkulu wa bungwe la FOCCAD Dan Nthara wati ndi okondwa ndi momwe anthuwa akuyendetsera ntchitozi, atapatsidwa mwayi osankha chitukuko chomwe akufuna m'dera lawo
Mkulu wa bungwe la FOKADI Dani Nthara wati ndi okondwa ndi momwe anthuwa akuyendetsera ntchitozi, atapatsidwa mwayi osankha chitukuko chomwe akufuna m'dera lawo
Female
Iye wati kwatsala tsopano ndikoti ntchitoyi ifikile midzi 24 m'bomali, pomwe pano, midzi 12 yokha ndiyomwe idachita mphumi
Iye wati kwatsala tsopano ndikoti ntchitoyi ifikile midzi twente folo m'bomali, pomwe pano, midzi twelofu yokha ndiyomwe idachita mphumi
Female
Ntchitoyi yomwe ikutchedwa "Titukulane" ikugwilidwa pansi pa ntchito yotchedwa Facilitated Community Action Programme m'chingerezi
Ntchitoyi yomwe ikutchedwa "Titukulane" ikugwilidwa pansi pa ntchito yotchedwa Fasilitetedi komyunite akishonu pulogalamu m'chingerezi
Female
pamodzi ndi bungwe la Spark MicroGrants ndi ndalama zosachepela k99 million. Nduna yowona zamasewero ndi achinyamata Uchizi Mkandawire
pamodzi ndi bungwe la Sipaki MayikloGilantsi ndi ndalama zosachepela nainte naini miliyoni kwacha. Nduna yowona zamasewero ndi achinyamata Uchizi Mkandawire
Female
lero ikhala nawo pa mwambo wapadera omwe akonzera timu ya mpira wa manja ya dziko lino ku Bingu International Conventions Center, BICC mu mzinda wa Lilongwe
lero ikhala nawo pa mwambo wapadera omwe akonzera timu ya mpira wa manja ya dziko lino ku Bingu Intaneshono konveshonzi senta Biayisisi mu mzinda wa Lilongwe
Female
yomwe ikhale ikupita m’dziko la South Africa ku mpikisano wa masewero a manja apa dziko lonse la pansi. Malingana ndi mlembi wa bungwe la Netball association of Malawi, NAM) Isaac Chimwala
yomwe ikhale ikupita m’dziko la Saufi afilika ku mpikisano wa masewero a manja apa dziko lonse la pansi. Malingana ndi mlembi wa bungwe la Netibo asosiyeshoni ofu Malawi, NAMU Aizeki Chimwala
Female
mwambowu awukonza kaamba koti nduna ya zamasewero Mkandawire, ikufuna kulimbikitsa osewera pomwe akhale akupita m’dziko la South Africa ku mpikisanowu
mwambowu awukonza kaamba koti nduna ya zamasewero Mkandawire, ikufuna kulimbikitsa osewera pomwe akhale akupita m’dziko la Saufi afilika ku mpikisanowu
Female
Iye wati, timu ya Queens yomwe pakadali pano ikuchita zokonzekera zake, inyamuka Lachisanu kupita mu mzinda wa Cape Town, m’dziko la South Africa
Iye wati, timu ya Kwinzi yomwe pakadali pano ikuchita zokonzekera zake, inyamuka Lachisanu kupita mu mzinda wa Kepi tauni, m’dziko la Saufi afilika
Komiti yaikulu pa khonsolo ya boma la Nkhotakota, lero yasankha khansala wa Bua wadi Charles Chimzukuzuku ngati mkhalapampando watsopano wa khonsoloyi, pa mkumano omwe ulimkati pakadalipano
Komiti yaikulu pa khonsolo ya boma la Nkhotakota, lero yasankha khansala wa Bua wadi Tchalosi Chimzukuzuku ngati mkhalapampando watsopano wa khonsoloyi, pa mkumano omwe ulimkati pakadalipano
Female
Iye walowa m’malo mwa Gaziel Chimzere wa Mpama wadi yemwe wakhala pa udindowu kwa telemu imodzi yokha. Chimzukuzuku komanso yemwe wasankhidwa ngati wachiwiri wake
Iye walowa m’malo mwa Gaziyelo Chimzere wa Mpama wadi yemwe wakhala pa udindowu kwa telemu imodzi yokha. Chimzukuzuku komanso yemwe wasankhidwa ngati wachiwiri wake
Female
Fiton Khofi wa boma wadi, asankhidwa opanda opikisana nawo. Phungu wanyumba yamalamulo wadera la ku mpoto m’bomali Henry Chimunthu Banda komanso wadera lapakati Peter Mazizi
Fitoni Khofi wa boma wadi, asankhidwa opanda opikisana nawo. Phungu wanyumba yamalamulo wadera la ku mpoto m’bomali Henele Chimunthu Banda komanso wadera lapakati Pita Mazizi
Female
ndi ena mwa omwe ali nawo pa mkumanowu. Bungwe la eni galimoto za mtundu wa minibus, laikira kumbuyo ganizo la ochita malonda agalimotozi lokweza mitengo yokwelera ma minibus
ndi ena mwa omwe ali nawo pa mkumanowu. Bungwe la eni galimoto za mtundu wa minibasi, laikira kumbuyo ganizo la ochita malonda agalimotozi lokweza mitengo yokwelera ma minibasi
Female
maka mchigawo chapakati m’dziko muno. Poyakhula ndi Umunthu FM, mlembi wa bungweli Coxley Kamange wati kukweza kwa mitengoku kwadza kaamba kakusowa kwa mafuta m’dziko muno
maka mchigawo chapakati m’dziko muno. Poyakhula ndi Umunthu efuemu, mlembi wa bungweli Cosile Kamange wati kukweza kwa mitengoku kwadza kaamba kakusowa kwa mafuta m’dziko muno
Female
Kamange wati akhala akukumana ndi boma kuti livomereze ganizo loti pazisungidwa malo amodzi omwe galimoto za mtundu wa minibus zizikamwetsa mafuta
Kamange wati akhala akukumana ndi boma kuti livomereze ganizo loti pazisungidwa malo amodzi omwe galimoto za mtundu wa minibus zizikamwetsa mafuta
Female
ndicholinga choti madalaivala asamayende mitunda yayitali kusaka mafuta munyengo yomwe mafuta akasowa, koma boma silikuchitapo kanthu pa ganizoli
ndicholinga choti madalaivala asamayende mitunda yayitali kusaka mafuta munyengo yomwe mafuta akasowa, koma boma silikuchitapo kanthu pa ganizoli
Female
Umunthu FM yapeza kuti maboma ena a mchigawo chapakati a Nkhotakota, Salima komanso Ntchisi ochita malonda agalimoto za mtundu wa minibus akweza mitengo yokwelera galimotozi
Umunthu efuemu yapeza kuti maboma ena a mchigawo chapakati a Nkhotakota, Salima komanso Ntchisi ochita malonda agalimoto za mtundu wa minibasi akweza mitengo yokwelera galimotozi
Female
Mlembi wa timu ya Silver Strikers Peter Masiye wati timu yake siyankhulapo kalikonse mpaka bungwe la SULOM litamaliza kafukufuku yemwe bungweli lakhazikikitsa
Mlembi wa timu ya siliva sitilaikazi Pita Masiye wati timu yake siyankhulapo kalikonse mpaka bungwe la SULOMU litamaliza kafukufuku yemwe bungweli lakhazikikitsa
Female
okhudza kupanga chinyengo pa masewero ndi timu ya Mighty Mukuru Wanderers. Mchikalata chomwe bungwe la SULOM lidatulutsa Lachiwiri, lidadzudzura matimu awiriwa
okhudza kupanga chinyengo pa masewero ndi timu ya Maite Mukuru Wandilazi. Mchikalata chomwe bungwe la SULOMU lidatulutsa Lachiwiri, lidadzudzura matimu awiriwa
Female
ati kaamba kopanga chinyengo maka pachiganizo chawo cholembera kalata limodzi yopempha kuti masewero amatimuwa omwe akuyenera kuchitika Lachinayi sabata ino awayimitse
ati kaamba kopanga chinyengo maka pachiganizo chawo cholembera kalata limodzi yopempha kuti masewero amatimuwa omwe akuyenera kuchitika Lachinayi sabata ino awayimitse
Female
Koma Masiye wauza Umunthu FM kuti iwo ndiodabwa kuti bungwe la SULOM likuonetsa ngati silikudziwapo kanthu pa nkhaniyi, pomwe matimuwa adakambiranaponso ndi akulu akulu ena pa nkhaniyi
Koma Masiye wauza Umunthu efuemu kuti iwo ndiodabwa kuti bungwe la SULOMU likuonetsa ngati silikudziwapo kanthu pa nkhaniyi, pomwe matimuwa adakambiranaponso ndi akulu akulu ena pa nkhaniyi
Female
Bungwe lothana ndi mchitidwe waziphuphu komanso katangale la ACB, lawonetsa kukhutira kuti mlandu omwe ukukhudza aphunzitsi anayi apakusukulu yakumudzi yosula maluso a manja
Bungwe lothana ndi mchitidwe waziphuphu komanso katangale la Esibi, lawonetsa kukhutira kuti mlandu omwe ukukhudza aphunzitsi anayi apakusukulu yakumudzi yosula maluso a manja
Female
ya Mbandira m’boma la Nkhotakota, omwe anamangidwa kaamba koganizilidwa kuti sanagwilitse bwino ntchito ndalama zapasukuluyi, ufika kumapeto posachedwapa
ya Mbandira m’boma la Nkhotakota, omwe anamangidwa kaamba koganizilidwa kuti sanagwilitse bwino ntchito ndalama zapasukuluyi, ufika kumapeto posachedwapa
Female
Poyankhula ndi Umunthu FM Lachiwiri ku bwalo la milandu la Nkhotakota Magistrate komwe mlanduwu ukumvedwa, mkulu ozenga milandu ku bungwe la ACB, Goda Lapozo
Poyankhula ndi Umunthu efuemu Lachiwiri ku bwalo la milandu la Nkhotakota Majesitileti komwe mlanduwu ukumvedwa, mkulu ozenga milandu ku bungwe la Esibi, Goda Lapozo
Female
wati mbali ya boma yabweretsa kale mboni zisanu ndipo yangotsala ndi mboni ziwiri pa nkhaniyi. Pomwe amavomeleza kuchedwa kwa mlanduwu, Lapozo wati mwa zina
wati mbali ya boma yabweretsa kale mboni zisanu ndipo yangotsala ndi mboni ziwiri pa nkhaniyi. Pomwe amavomeleza kuchedwa kwa mlanduwu, Lapozo wati mwa zina
Female
izi ndi kaamba ka nthawi yomwe imatengedwa pofunsa mboni. M’mwezi wa Epulo chaka chatha, bungwe la ACB linamanga aphunzitsi anayiwa omwe ndi Jomo Chimfomboti, Alinafe Wane
izi ndi kaamba ka nthawi yomwe imatengedwa pofunsa mboni. M’mwezi wa Epulo chaka chatha, bungwe la Esibi linamanga aphunzitsi anayiwa omwe ndi Jomo Chimfomboti, Alinafe Wane
Female
Eddington Kaudzu komanso Mike Maseya, bungweri litalandira dandaulo kuti anagula katundu wa ndalama zokwana K3.5 million m’malo mwa katundu wa ndalama zokwana K10 million
Eding’itoni Kaudzu komanso Maiki Maseya, bungweri litalandira dandaulo kuti anagula katundu wa ndalama zokwana fili pointi faifi miliyoni kwacha m’malo mwa katundu wa ndalama zokwana Teni miliyonii kwacha
Female
ndipo anagawana ndalama zokwana K6.5 million pa unayi wawo. Mkulu ozenga milandu wa boma, Masauko Chamkakala watsimikiza kuti walembera bwalo la milandu la High Court ku Blantyre
ndipo anagawana ndalama zokwana sikisi pointi faifi miliyoni kwacha pa unayi wawo. Mkulu ozenga milandu wa boma, Masauko Chamkakala watsimikiza kuti walembera bwalo la milandu la Hai khoti ku Bulantaya
Female
kuti limasule mtsogoleri wakale wa dziko lino, Dr Bakali Muluzi pa milandu yonse yomwe amayankha kwa zaka 14 tsopano
kuti limasule mtsogoleri wakale wa dziko lino, Dokota Bakali Muluzi pa milandu yonse yomwe amayankha kwa zaka fotini tsopano
Female
Dr Muluzi amayankha mlandu okhudza kusagwilitsa bwino ntchito ndalama zamisonkho ya a Malawi zokwana K1.7 billion
Dokota Muluzi amayankha mlandu okhudza kusagwilitsa bwino ntchito ndalama zamisonkho ya a Malawi zokwana wani pointi seveni miliyoni kwacha
Female
Chamkakala wauza Umunthu FM kuti mwa zina, aganiza zothetsa mlanduwu poganizira kuti boma lawononga ndalama zochuluka pa mlanduwu, pomwe mboni zina pa nkhaniyi
Chamkakala wauza Umunthu Efuemu kuti mwa zina, aganiza zothetsa mlanduwu poganizira kuti boma lawononga ndalama zochuluka pa mlanduwu, pomwe mboni zina pa nkhaniyi
Female
zinasokonekera komanso kumwalira kumene. Iye wati atawunikira chitsogolo cha nkhaniyi, aganiza zongothetsa mlanduwu pofuna kusamala ndalama za misonkho ya a Malawi
zinasokonekera komanso kumwalira kumene. Iye wati atawunikira chitsogolo cha nkhaniyi, aganiza zongothetsa mlanduwu pofuna kusamala ndalama za misonkho ya a Malawi
Female
Komabe, Chamkakala wati apeleka lipoti latsatanetsatane lokhudza nkhaniyi ku nyumba yamalamulo. Pakadalipano, Dr Muluzi alibe mlandu ulionse oti ayankhe okhudza nkhaniyi
Komabe, Chamkakala wati apeleka lipoti latsatanetsatane lokhudza nkhaniyi ku nyumba yamalamulo. Pakadalipano, Dokota Muluzi alibe mlandu ulionse oti ayankhe okhudza nkhaniyi
Female
pomwe m’mawa wa lero, bwalo la High Court ku Blantyre lathetsa mlanduwu. M'modzi wawombeledwa, apolisi atatu avulazidwa pa ADMARC ya Bua ku Nkhotakota
pomwe m’mawa wa lero, bwalo la Hayi khoti ku Bulantaya lathetsa mlanduwu. M'modzi wawombeledwa, apolisi atatu avulazidwa pa ADIMAKI ya Buwa ku Nkhotakota
Female
Ku m'mawaku, mnyamata wina yemwe akudziwika bwino ndi dzina loti Mbewe wavulazidwa, chipolopolo chomwe ati chinawombeledwa m'mwamba pa nthawi yomwe amamenyana ndi wapolisi chitamugwera pa mwendo
Ku m'mawaku, mnyamata wina yemwe akudziwika bwino ndi dzina loti Mbewe wavulazidwa, chipolopolo chomwe ati chinawombeledwa m'mwamba pa nthawi yomwe amamenyana ndi wapolisi chitamugwera pa mwendo
Female
Malingana ndi wachiwiri kwa mkulu wa polisi ya Nkhotakota Surpritendent Clement Mwale, kutsatira kusamvana ndi wapolisi yemwe amakhazikitsa bata pa nthawi yomwe anthu amagula chimanga pa ADMARC-yi
Malingana ndi wachiwiri kwa mkulu wa polisi ya Nkhotakota Supulitendanti Kilementi Mwale, kutsatira kusamvana ndi wapolisi yemwe amakhazikitsa bata pa nthawi yomwe anthu amagula chimanga pa ADIMAKI-yi
Female
Mbewe anayamba kumenyana ndi wapolisiyu kenako amafuna kulanda mfuti, koma poziteteza, wapolisiyu anawombela m'mwamba ndipo pobwelera chipolopolo chinamugwera pa mwendo ndipo wavulala
Mbewe anayamba kumenyana ndi wapolisiyu kenako amafuna kulanda mfuti, koma poziteteza, wapolisiyu anawombela m'mwamba ndipo pobwelera chipolopolo chinamugwera pa mwendo ndipo wavulala
Female
Mwale wati kupezeka kwa apolisi pa ADMAC-yi kunali kufuna kuwonesetsa kuti mavenda sakulowelera ntchito yogula chimanga pamalowa. Iye wati kutsatira chipwilikiti chomwe chinabuka pa nthawiyi
Mwale wati kupezeka kwa apolisi pa ADIMAKI-yi kunali kufuna kuwonesetsa kuti mavenda sakulowelera ntchito yogula chimanga pamalowa. Iye wati kutsatira chipwilikiti chomwe chinabuka pa nthawiyi
Female
apolisi anathila utsi okhetsa msozi anthu atayamba kuwamenya, ndipo atatu kuphatikiza mkulu oyang'anira polisi yaing'ono ya Mpondagaga avulazidwa
apolisi anathila utsi okhetsa msozi anthu atayamba kuwamenya, ndipo atatu kuphatikiza mkulu oyang'anira polisi yaing'ono ya Mpondagaga avulazidwa
Female
ndipo akulandila thandizo la mankhwara pa chipatara cha Nkhotakota. Koma ena mwa anthu omwe anawona izi zikuchitika, ati wapolisi oyamba anamenya Mbewe m'mutu ndi mfuti
ndipo akulandila thandizo la mankhwara pa chipatara cha Nkhotakota. Koma ena mwa anthu omwe anawona izi zikuchitika, ati wapolisi oyamba anamenya Mbewe m'mutu ndi mfuti
Female
ndipo anakalandila thandizo kuchipatara komwe anakamusoka, kenako anabwelera nkupezaso wapolisi wina yemwe anayambaso kumenyana naye
ndipo anakalandila thandizo kuchipatara komwe anakamusoka, kenako anabwelera nkupezaso wapolisi wina yemwe anayambaso kumenyana naye
Female
Mkati momenyana, wapolisi winayu anawombela katatu, kamodzi m'mwamba, kamodzi pansi kenako anawombela pa mwendo wa Mbewe yemwe amafuna kulanda mfuti
Mkati momenyana, wapolisi winayu anawombela katatu, kamodzi m'mwamba, kamodzi pansi kenako anawombela pa mwendo wa Mbewe yemwe amafuna kulanda mfuti
Female
osati m'mwamba ngati momwe apolisi akunenera, ndipo akulandilaso thandizo pachipatara cha Nkhotakota. Pakadalipano, bata la bwelera pa malowa koma ntchito yogulitsa chimanga yayamba yaimitsidwa kaye
osati m'mwamba ngati momwe apolisi akunenera, ndipo akulandilaso thandizo pachipatara cha Nkhotakota. Pakadalipano, bata la bwelera pa malowa koma ntchito yogulitsa chimanga yayamba yaimitsidwa kaye
Female
Nthambi yowona zanyengo ndikusintha kwa nyengo m’dziko muno, yati ipitiliza kulondola kayendedwe ndi nyonga za Namondwe otchedwa DUMAKO, yemwe wabuka pa nyanja ya India
Nthambi yowona zanyengo ndikusintha kwa nyengo m’dziko muno, yati ipitiliza kulondola kayendedwe ndi nyonga za Namondwe otchedwa DUMAKO, yemwe wabuka pa nyanja ya Indiya
Female
Pakadali pano, Namondweyu akuyenda molunjika chilumba cha Madagascar pa liwiro la makilomita 20 pa ola
Pakadali pano, Namondweyu akuyenda molunjika chilumba cha Madagasika pa liwiro la makilomita tuwente pa ola
Female
ndipo akachoka pachilumba cha Madagascar, DUMAKO atha kulowa pa Nyanja ya mchere ya pakati pa Madagascar ndi dziko la Mozambique
ndipo akachoka pachilumba cha Madagasika, DUMAKO atha kulowa pa Nyanja ya mchere ya pakati pa Madagasika ndi dziko la Mozambiki
Female
Malingana ndi chikalata chomwe nthambiyi yatulutsa lero, pamene ali pano, Namondwe otchedwa DUMAKO sakukhudzana ndi nyengo kapena kagwedwe ka Mvura mu dziko la Malawi
Malingana ndi chikalata chomwe nthambiyi yatulutsa lero, pamene ali pano, Namondwe otchedwa DUMAKO sakukhudzana ndi nyengo kapena kagwedwe ka Mvura mu dziko la Malawi
Female
Nthambiyi yati, ndikofunikila kuzindikila kuti nyengo ya dzinja ndi nyengonso ya a namondwe ndipo pafupifupi a namondwe oposela asanu ndi anayi
Nthambiyi yati, ndikofunikila kuzindikila kuti nyengo ya dzinja ndi nyengonso ya a namondwe ndipo pafupifupi a namondwe oposela asanu ndi anayi
Female
amakhala akubadwa munyanja ya mchere koma ena mwaiwo amathelamo osakhudza nyengo ya dziko la Malawi. Nduna yowona za ntchito Vera Kamtukule yati, undunawu uchititsa msonkhano wa oremba nkhani posachedwapa
amakhala akubadwa munyanja ya mchere koma ena mwaiwo amathelamo osakhudza nyengo ya dziko la Malawi. Nduna yowona za ntchito Vera Kamtukule yati, undunawu uchititsa msonkhano wa oremba nkhani posachedwapa
Female
komwe akafotokoze bwino momwe boma lakwanitsira kuremba ntchito achinyamata okwana 997, 423 mchaka cha chuma cha boma cha 2021/2022
komwe akafotokoze bwino momwe boma lakwanitsira kuremba ntchito achinyamata okwana naini handiledi andi nainte seveni folo handiledi andi twente fili mchaka cha chuma cha boma cha twente twente wani twente twente thu
Female
Pomwe Umunthu FM imafuna kumva kwa ndunayi, momwe boma lapezera chiwerengero cha achinyamata omwe arembedwa ntchitowa, Kamtukule wati, a Malawi adzafotokozeledwa bwino za nkhaniyi Lolemba sabata lamawa
Pomwe Umunthu efuemu imafuna kumva kwa ndunayi, momwe boma lapezera chiwerengero cha achinyamata omwe arembedwa ntchitowa, Kamtukule wati, a Malawi adzafotokozeledwa bwino za nkhaniyi Lolemba sabata lamawa
Female
Poyankhura m'nyumba yamalamulo Lachinayi, mtsogoleri wa dziko lino Dr Chakwera anati boma lakwanitsa kuremba ntchito achinyamatawa ngakhare panali mavuto omwe anasautsa zedi monga matenda a Korona
Poyankhura m'nyumba yamalamulo Lachinayi, mtsogoleri wa dziko lino Dokota Chakwera anati boma lakwanitsa kuremba ntchito achinyamatawa ngakhare panali mavuto omwe anasautsa zedi monga matenda a Korona
Female
Koma, izi zadzetsa zoyankhura zochuluka pakati pa a Malawi, pomwe ena akuti ndi momwe zinthu zilili pakadalipano, ndikulakwa kuti boma liti lalemba ntchito achinyamata ochuluka motere
Koma, izi zadzetsa zoyankhura zochuluka pakati pa a Malawi, pomwe ena akuti ndi momwe zinthu zilili pakadalipano, ndikulakwa kuti boma liti lalemba ntchito achinyamata ochuluka motere
Female
Pakadalipano, bungwe la achinyamata la Mzuzu City Youth Caucus, lapempha mtsogoleri wa dziko lino kuti abwere poyera nkufotokozera mtundu wa a Malawi
Pakadalipano, bungwe la achinyamata la Mzuzu site yufi kakasi, lapempha mtsogoleri wa dziko lino kuti abwere poyera nkufotokozera mtundu wa a Malawi
Female
momwe boma lapezera chiwerengerochi, komwe achinyamatawa akugwilira ntchito komanso afotokozere dziko lino tsatanetsatane wa achinyamata omwe arembedwa ntchitowa
momwe boma lapezera chiwerengerochi, komwe achinyamatawa akugwilira ntchito komanso afotokozere dziko lino tsatanetsatane wa achinyamata omwe arembedwa ntchitowa
Female
Nthambi yowona zanyengo ndikusintha kwa nyengo m’dziko muno, yati dziko lino likuyembekezereka kukhalabe likulandira nyengo yotentha ndipo nyengoyi, ipitilila kukhala chonchi kwa masiku asanu akubwerawa
Nthambi yowona zanyengo ndikusintha kwa nyengo m’dziko muno, yati dziko lino likuyembekezereka kukhalabe likulandira nyengo yotentha ndipo nyengoyi, ipitilila kukhala chonchi kwa masiku asanu akubwerawa
Female
Malingana ndi uthenga okhudza zanyengo omwe nthambiyi imatulutsa tsiku lililonse, madera ambiri, alandira nyengo yotentha kwabasi yopitirira pa 4 Degree Celsus
Malingana ndi uthenga okhudza zanyengo omwe nthambiyi imatulutsa tsiku lililonse, madera ambiri, alandira nyengo yotentha kwabasi yopitirira pa folo digili seshazi
Female
Chenjezo: Malingana ndi nyengo yotenthayi, nthambi yowona za nyengo, ikuchenjeza anthu onse kuti azikhala ndi madzi akumwa ozizila bwino, komanso apewe kukhala pa mtetete pa dzuwa
Chenjezo: Malingana ndi nyengo yotenthayi, nthambi yowona za nyengo, ikuchenjeza anthu onse kuti azikhala ndi madzi akumwa ozizila bwino, komanso apewe kukhala pa mtetete pa dzuwa
Female
makamaka pakati pa nthawi ya 12 koloko masana ndi 3 koloko masana chifukwa pa nthawiyi, ndipomwe kunja kukumakhala kwadzuwa lambili. Khalani ochenjera, khalani odziwa zanyengo
makamaka pakati pa nthawi ya twelofu koloko masana ndi fili koloko masana chifukwa pa nthawiyi, ndipomwe kunja kukumakhala kwadzuwa lambili. Khalani ochenjera, khalani odziwa zanyengo
Female
Msonkhano wa akuluakulu a khonsolo ya mu mzinda wa Zomba " Full Council Meeting wathera panjira lero lolemba kamba kosamvana pakati pa makhansala ndi mfumu ya munzindawu a Davie Maunde
Msonkhano wa akuluakulu a khonsolo ya mu mzinda wa Zomba " Fu khanso miting’i wathera panjira lero lolemba kamba kosamvana pakati pa makhansala ndi mfumu ya munzindawu a Devi Maunde
Female
Izi zikudzaso pamene msonkhano ngati omweu udalephelekaso la Chisanu pa 2 february chifukwa chakuti mfumu ya mzindawu a Maunde
Izi zikudzaso pamene msonkhano ngati omweu udalephelekaso la Chisanu pa Thu febuluwale chifukwa chakuti mfumu ya mzindawu a Maunde
Female
ndi a chiwiri awo a Munira Bakali adapita ku Lilongwe komwe kumachitika masewero a mpira a Chikho cha FDH intercity Mayor's Trophy
ndi a chiwiri awo a Munira Bakali adapita ku Lilongwe komwe kumachitika masewero a mpira a Chikho cha Efudietchi intasite meyazi thilofe
Female
Poyakhula ndi khansala wa mpira ward a Christopher Jana ati pofuna kulepheletsa Full Council Meeting pafunika kutsatira ndondomeko osangonena ndi pakamwa
Poyakhula ndi khansala wa mpira wadi a khilisitofa Jana ati pofuna kulepheletsa "Fukhanso miting’i pafunika kutsatira ndondomeko osangonena ndi pakamwa
Female
Iwo ati a Mayor ndi omwe alepheletsa msonkhanoso kamba koti zomwe anawaitanila lero panalibe pa ma Agenda, ati sangatenge zithu zina za la chisanu pa 2 February kuti akambirane lero pa 5 February
Iwo ati a Meya ndi omwe alepheletsa msonkhanoso kamba koti zomwe anawaitanila lero panalibe pa ma Ajenda, ati sangatenge zithu zina za la chisanu pa thu febuluwale kuti akambirane lero pa faifi febuluwale
Female
Ati a Mayor akanakhala kuti akupanga zithu mwadongosolo akanafotokozera anthu anali mu Chamber zifukwa zomwe adalepheletsa msonkhano Full Council Meeting
Ati a Meya akanakhala kuti akupanga zithu mwadongosolo akanafotokozera anthu anali mu Chamber zifukwa zomwe adalepheletsa msonkhano Fukhanso miting’i
Female
wa pa 2 february Lachisanu koma poti utsogoleri wawo ndiwakuti ndanena ndanena atero a Jana. Ndipo poyakhulapo Mfumu ya mu mzindawu a Maunde
wa pa thu febuluwale Lachisanu koma poti utsogoleri wawo ndiwakuti ndanena ndanena atero a Jana. Ndipo poyakhulapo Mfumu ya mu mzindawu a Maunde
Female
ati makhansala a Chipani Cha DPP ati ndiomwe asokoneza msonkhano wa lero. kusowa kwa ndalama za mayiko ena m'dziko muno kukupitilira kukhudza nkhani za malonda
ati makhansala a Chipani Cha DIPIPI ati ndiomwe asokoneza msonkhano wa lero. kusowa kwa ndalama za mayiko ena m'dziko muno kukupitilira kukhudza nkhani za malonda
Female
watero m'modzi Mwa M'zika za dziko lino kuchokera m'boma la Lilongwe, Gloria Kamwendo. Kamwendo yemwe ndi mwini mashopu odziwika ndi dzina loti Delightful Deliveries
watero m'modzi Mwa M'zika za dziko lino kuchokera m'boma la Lilongwe, Guloliya Kamwendo. Kamwendo yemwe ndi mwini mashopu odziwika ndi dzina loti Delaitifu delivalezi
Female
amachita malonda ogulitsa zipangizo zomwe zimaperekedwa mu nthawi ya zikondwerero ndipo mwa zina ndi Maluwa,Mafuta onukhulitsa komanso zokometsera maonekedwa
amachita malonda ogulitsa zipangizo zomwe zimaperekedwa mu nthawi ya zikondwerero ndipo mwa zina ndi Maluwa,Mafuta onukhulitsa komanso zokometsera maonekedwa
Female
watsimikiza izi mu mzinda wa Blantyre la Chisanu potsegulira nyumba yake yogulitsira katundu. Iye wati vutoli likuchititsa kuti Katundu akaodedwa kuchokera kuja kwa dziko lino
watsimikiza izi mu mzinda wa Bulantaya la Chisanu potsegulira nyumba yake yogulitsira katundu. Iye wati vutoli likuchititsa kuti Katundu akaodedwa kuchokera kuja kwa dziko lino
Female
azichedwa kufika m'dziko muno zomwe zikuchititsa ogula kutaya chikhulupiriro pa kapezedwe kake, choncho boma lilingalire izi mwapadera
azichedwa kufika m'dziko muno zomwe zikuchititsa ogula kutaya chikhulupiriro pa kapezedwe kake, choncho boma lilingalire izi mwapadera
Female
Ndipo m'mawu ake,m'modzi mwa anthu omwe anafika Ku mwambowu mu mzinda wa Blantyre, Madonna Banda wati mitengo yake ndiyotsika bwino choncho malondawa afika mu nthawi yake
Ndipo m'mawu ake,m'modzi mwa anthu omwe anafika Ku mwambowu mu mzinda wa Bulantaya, Madona Banda wati mitengo yake ndiyotsika bwino choncho malondawa afika mu nthawi yake
Female
pomwe pa 14 February maiko akhale akukondwerera valentine day yomwe ndi nkhani ya Chikondi. Iyi ikhala shop yoyamba mu mzinda wa Blantyre komanso yachiwiri m'dziko muno pomwe yoyamba ili mu mzinda wa Lilongwe
pomwe pa fotini febuluwale maiko akhale akukondwerera valentaini deyi yomwe ndi nkhani ya Chikondi. Iyi ikhala shopu yoyamba mu mzinda wa Bulantaya komanso yachiwiri m'dziko muno pomwe yoyamba ili mu mzinda wa Lilongwe
Female
Panali kusamvana pakati pa ma khansala, adindo ndi Mayor wa mu mzinda wa Zomba, Khansala Davie Maunde kamba kakulepheletsa kwa Full Council Meeting dzulo
Panali kusamvana pakati pa ma khansala, adindo ndi Meya wa mu mzinda wa Zomba, Khansala Devi Maunde kamba kakulepheletsa kwa fukhanso miting’i dzulo
Female
Malingana ndi modzi mwama khansala a Christoper Jana a mpira ward ati amayenela kukhala ndi full Council meeting dzulo
Malingana ndi modzi mwama khansala a Khilisitofa Jana a mpira wadi ati amayenela kukhala ndi fukhanso miting’i dzulo
Female
ndipo adadziwitsidwa masiku apitawo ndipo aliyense adabwera ku full Council meeting. Koma chodabwitsa ndi chakuti a mfumu ya mu mzindawu ndi wachiwiri wake kunalibeko
ndipo adadziwitsidwa masiku apitawo ndipo aliyense adabwera ku fukhanso miting’i. Koma chodabwitsa ndi chakuti a mfumu ya mu mzindawu ndi wachiwiri wake kunalibeko
Female