audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Ena mwa oimba akunjawa ndi Alaine, Yo Maps, ndi Blaq Diamond komaso oimba wa kuno ku Malawi Kell Kay. Anthu opitilira 20,000 ndiomwe akuyembekezereka kuzapezeka pa mwambowu
Ena mwa oimba akunjawa ndi Aleni, Yo Mapsi, ndi Bulaki Dayamondi komaso oimba wa kuno ku Malawi Kewo keyi. Anthu opitilira twente sauzande ndiomwe akuyembekezereka kuzapezeka pa mwambowu
Female
Katswili osewera kutsogolo mutimu ya Ascent Academy yemwe amasewera kutimu ya Blue Eagles pangongole, Christopher Gototo
Katswili osewera kutsogolo mutimu ya Asenti akadame yemwe amasewera kutimu ya Buli Igozi pangongole, Khilisofa Gototo
Female
akuyembekezereka kusaina kutimu ya Silver Strikers kumathero kwa sabata ino. Ife, tapeza kuti timu ya Silver Strikers ikukambirana ndi Ascent ndipo kumathero kwa sabata ino
akuyembekezereka kusaina kutimu ya siliva sitilaikazi kumathero kwa sabata ino. Ife, tapeza kuti timu ya siliva sitilaikazi ikukambirana ndi Asenti ndipo kumathero kwa sabata ino
Female
akhala atamaliza kumvana ndipo osewerayu atumikira mu central bankers. Timu ya Ascent inalembera Blue Eagles kuti ipereka ndalama zokwana Five Million Malawi Kwacha
akhala atamaliza kumvana ndipo osewerayu atumikira mu sentilo bankazi. Timu ya Asenti inalembera Bulu igozi kuti ipereka ndalama zokwana faifi miliyoni Malawi Kwacha
Female
kuti igure osewera kutsogolo yemwe anawagolesera zigoli zisanuyu koma sanamvane bwino bwino. Iye asanabwere kutimu ya Blue Eagles, anatumikirapo kutimu ya Sable Farming
kuti igure osewera kutsogolo yemwe anawagolesera zigoli zisanuyu koma sanamvane bwino bwino. Iye asanabwere kutimu ya Bulu igozi, anatumikirapo kutimu ya Sebo Faming’i
Female
Mighty Mukuru Wanderers yagula timu ya mpira wa miyendo koma osewera ake kukhala atsikana women's football ya Bangwe Super Queen women's football
Maite Mukuru Wandilazi yagula timu ya mpira wa miyendo koma osewera ake kukhala atsikana wimenzi futubo ya Bangwe supa kwinzi wimenzi futubo
Female
ndipo timu yi yasitha. Ndipo izitchedwa Mighty Mukuru Wanderers Women's football. Timu ya Dedza Dynamos Salima Sugar FC tsopano yatenga Gilbert Chirwa
ndipo timu yi yasitha. Ndipo izitchedwa Maite Mukuru wandilazi wimenzi futubo. Timu ya Dedza Dainamozi Salima shuga efusi tsopano yatenga Gilibati Chirwa
Female
kukhala mphunzitsi wao wamkulu kutsatira kuchoka kwa Dan Dzikambani. Malinga ndizomwe zalembedwa pa tsamba la mchezo la Facebook latimuyu, tate wakale ophunzitsa timu ya Ekwendeni Hammers yu
kukhala mphunzitsi wao wamkulu kutsatira kuchoka kwa Dani Dzikambani. Malinga ndizomwe zalembedwa pa tsamba la mchezo la Fesibuku latimuyu, tate wakale ophunzitsa timu ya Ekwendeni Hamazi yu
Female
wafika ku Dedza ndipo agwilizana zonse zofunika. Iye wapasidwaso mwai kuti asankhe ekha wachiwili wake oti azithandizana kuphunzitsa timuyi
wafika ku Dedza ndipo agwilizana zonse zofunika. Iye wapasidwaso mwai kuti asankhe ekha wachiwili wake oti azithandizana kuphunzitsa timuyi
Female
kuphatikizapo Christopher Zinyongo yemwe akhalabe kutimuyi ngati m'modzi wa aphunzitsi othandizira timuyi
kuphatikizapo khilisitofa Zinyongo yemwe akhalabe kutimuyi ngati m'modzi wa aphunzitsi othandizira timuyi
Female
Kutsatira mphekesera zomwe tapeza, zikuonetsa kuti Dan Zimkambani sakhalaso mphunzitsi wamkulu watimu ya Dedza Dynamos Salima Sugar FC chaka chino cha 2023
Kutsatira mphekesera zomwe tapeza, zikuonetsa kuti Dani Zimkambani sakhalaso mphunzitsi wamkulu watimu ya Dedza Dainamozi Salima Shuga efusi chaka chino cha twente twente fili
Female
pomwe league yaikulu m'dziko muno ikhale ikuyamba mwezi wamawa. Izi zili momwemu kutsatira ndondomeko ya Club License yoti mphunzitsi wamkulu akuyenera kukhala ndi pepala la CAF B
pomwe ligi yaikulu m'dziko muno ikhale ikuyamba mwezi wamawa. Izi zili momwemu kutsatira ndondomeko ya kilabu laisensi yoti mphunzitsi wamkulu akuyenera kukhala ndi pepala la KAFU Bi
Female
kuti aphunzitse timu ndipo Dan Zimkambani alibe pepala limeneli. Ife tapeza kuti akuluakulu atimuyi anali ndi mkumano dzulo, ndipo amvana zoti apeze wina oti alowe m'malo mwa Dan
kuti aphunzitse timu ndipo Dani Zimkambani alibe pepala limeneli. Ife tapeza kuti akuluakulu atimuyi anali ndi mkumano dzulo, ndipo amvana zoti apeze wina oti alowe m'malo mwa Dani
Female
Dzina la mphunzitsi wamkulu watimu ya Ekwendeni Hammers, Gilbert Chirwa ndi lomwe latchulidwa kwambiri kuti apite ku Dedza Dynamos Salima Sugar FC
Dzina la mphunzitsi wamkulu watimu ya Ekwendeni Hamazi, Gilibati Chirwa ndi lomwe latchulidwa kwambiri kuti apite ku Dedza Dainamozi Salima Shuga efusi
Female
Khonsolo ya boma la Zomba yavomeleza ndondomeko ya Za chuma yokwana 28 billion ya Chaka chino 2023 mpana 2024
Khonsolo ya boma la Zomba yavomeleza ndondomeko ya Za chuma yokwana twente eiti biliyoni ya Chaka chino twente twente fili mpana twente twente folo
Female
Mwa Zina budget yi muli ntchito za Umoyo za Ma phunziro, Za ulimi, Za Achinyamata ndi zina zotero. Bwana nkubwa wa boma la Zomba a Reignard Chavula
Mwa Zina bajeti yi muli ntchito za Umoyo za Ma phunziro, Za ulimi, Za Achinyamata ndi zina zotero. Bwana nkubwa wa boma la Zomba a Reinadi Chavula
Female
ati budget yi ikupeleka chikhulupilira kwa anthu aku zomba, Ndipo ati muli ntchito zosiyana siyana zomwe zipangise kut anthu aku Zomba apindule ndi budget imeneneyi
ati bajeti yi ikupeleka chikhulupilira kwa anthu aku zomba, Ndipo ati muli ntchito zosiyana siyana zomwe zipangise kut anthu aku Zomba apindule ndi bajeti imeneneyi
Female
A Police a Ku Zomba amanga ophunzila apa Sukulu ya Secondary ya Malosa okwana 70. kamba kokhunzidwa ndi Zionesero zomwe zachitika pa Sukulupo
A Police a Ku Zomba amanga ophunzila apa Sukulu ya Sekondale ya Malosa okwana sevente. kamba kokhunzidwa ndi Zionesero zomwe zachitika pa Sukulupo
Female
Ofalisa khani Za a police ku Zomba Patricia Supiliano atsimikiza za khaniyi poyakhula ndi wailesi ya Ufulu
Ofalisa khani Za a polisi ku Zomba Paatilisha Supiliyano atsimikiza za khaniyi poyakhula ndi wailesi ya Ufulu
Female
Ophunzilawa anayambisa Zionesero kamba kosamvana ndi Akulu Akulu a pa Sukulupo. Atawachosa ophunzira awiri atapezeka akusuta Chamba
Ophunzilawa anayambisa Zionesero kamba kosamvana ndi Akulu Akulu a pa Sukulupo. Atawachosa ophunzira awiri atapezeka akusuta Chamba
Female
Ndipo Mwa ophunzira 70 omwe amangidwawo 6 ndiomwe amasogolera Zionetsero . Popitiliza ntchito yomwe akhala akuchita, Platinum Fitness
Ndipo Mwa ophunzira sevente omwe amangidwawo sikisi ndiomwe amasogolera Zionetsero. Popitiliza ntchito yomwe akhala akuchita, Pulatinamu fitinesi
Female
yakonzaso masewero amajowajowa olimbitsa matupi omwe achitike lachisanu pa 3 March 2023 tsiku la tchuthi
yakonzaso masewero amajowajowa olimbitsa matupi omwe achitike lachisanu pa fili machi twente twente fili tsiku la tchuthi
Female
Mkulu wa Platinum Fitness Ndaona M'bwana, wati akufuna kupitiliza cholinga chao chofuna anthu ambiri kuti akhale ndi matupi athanzi
Mkulu wa pulatinamu fitinesi Ndaona M'bwana, wati akufuna kupitiliza cholinga chao chofuna anthu ambiri kuti akhale ndi matupi athanzi
Female
onenepa kopyola muyezo akachepese matupi awo ndipo zonsezi zichitika ku Kamuzu Institute for Sports ku Lilongwe
onenepa kopyola muyezo akachepese matupi awo ndipo zonsezi zichitika ku Kamuzu insichuti ofu sipotsi ku Lilongwe
Female
Mumawu ake M'bwana anapitiliza ndikunena kuti kupatura majowajowa omwe akayambe nthawi ya 6 koloko mamawa, akakhalaso ndi nthawi yowaunikira anthu omwe akafike ku Kamuzu Institute for Sports
Mumawu ake M'bwana anapitiliza ndikunena kuti kupatura majowajowa omwe akayambe nthawi ya sikisi koloko mamawa, akakhalaso ndi nthawi yowaunikira anthu omwe akafike ku Kamuzu insichuti ofu sipotsi
Female
Zokhuza kapewedwe ka nthenda ya Cholera. Aliyense ozatenga nawo gawo pa tsikuli akuyenera kudzalipira ndalama yokwana K2000
Zokhuza kapewedwe ka nthenda ya kolela. Aliyense ozatenga nawo gawo pa tsikuli akuyenera kudzalipira ndalama yokwana thu sauzande kwacha
Female
Ophunzira apa Sukulu ya Secondary ya Malosa atetha sukulu kamba kosamvana ndi Akulu Akulu apa sukulupo
Ophunzira apa Sukulu ya Sekondale ya Malosa atetha sukulu kamba kosamvana ndi Akulu Akulu apa sukulupo
Female
Malingani ndi mneneri wa Police ku Zomba Patricia Supiliano ati ophunzila awiri apasukulupo anapezeka akusuta Chamba. Zomwe ndi zosephana ndi Malamulo apa Sukulupo
Malingani ndi mneneri wa Polisi ku Zomba Patilisha Supiliano ati ophunzila awiri apasukulupo anapezeka akusuta Chamba. Zomwe ndi zosephana ndi Malamulo apa Sukulupo
Female
Mwa izi akulu akulu apa Sukulupo anawachosa anawa zomwe zinapangitsa kuti ana enawo akwiye nkuyamba Zionesero pa Sukulupo
Mwa izi akulu akulu apa Sukulupo anawachosa anawa zomwe zinapangitsa kuti ana enawo akwiye nkuyamba Zionesero pa Sukulupo
Female
Mwa izi akulu akulu apa Sukulupo anawachosa anawa zomwe zinapangitsa kuti ana enawo akwiye nkuyamba Zionesero pa Sukulupo
Mwa izi akulu akulu apa Sukulupo anawachosa anawa zomwe zinapangitsa kuti ana enawo akwiye nkuyamba Zionesero pa Sukulupo
Female
Mwazina ophunzirawa atetha Generator , kalasi yophunzilirapo maphunziro a Science ndi Ma ofesi
Mwazina ophunzirawa atetha jeneleta , kalasi yophunzilirapo maphunziro a sayansi ndi Ma ofesi
Female
Unduna Wa za umoyo watsutsa zoti ukupereka ndalama kudzera mmafoni ngati nthandizo kwa anthu kutsatira kubuka kwa nthenda ya Cholera komanso Covid-19, mdziko muno
Unduna Wa za umoyo watsutsa zoti ukupereka ndalama kudzera mmafoni ngati nthandizo kwa anthu kutsatira kubuka kwa nthenda ya Cholera komanso kovidi - naintini, mdziko muno
Female
Mlembi wa mkulu ku Unduna wa za umoyo a Charles Mwansambo atsimikiza izi kudzera mu kalata yomwe undunawu watulutsa
Mlembi wa mkulu ku Unduna wa za umoyo a Tchalosi Mwansambo atsimikiza izi kudzera mu kalata yomwe undunawu watulutsa
Female
Kalatayi yabweretsa poyera zomwe anthu ena a ukamberembere akuchita potumizira anthu mauthenga a bodza apa foni kuti atumizilidwa ndalama ndi boma
Kalatayi yabweretsa poyera zomwe anthu ena a ukamberembere akuchita potumizira anthu mauthenga a bodza apa foni kuti atumizilidwa ndalama ndi boma
Female
kudzera mu undunawu pa lamya ndipo kuti ayimbe pagwiritsa ntchito nambala zachilendo kuti alandire ndalamazo
kudzera mu undunawu pa lamya ndipo kuti ayimbe pagwiritsa ntchito nambala zachilendo kuti alandire ndalamazo
Female
Apa unduna wa za umoyowu wapemba kampani za lamya mothandizana ndi apolisi kuti athane ndi akamberemberewa popanga nambalazi kuti zisapitilire kugwira ntchito
Apa unduna wa za umoyowu wapemba kampani za lamya mothandizana ndi apolisi kuti athane ndi akamberemberewa popanga nambalazi kuti zisapitilire kugwira ntchito
Female
Katswili osewera mutimu ya Dedza Dynamos Charles Chipala, ali m'dziko la Mozambique komwe akuyesa mwai kutimu ya UD Songo
Katswili osewera mutimu ya Dedza Dainamozi Tchalosi Chipala, ali m'dziko la Mozambiki komwe akuyesa mwai kutimu ya yudi Songo
Female
Katswiliyu waonedwa ali ndi mtsogoleri wa osewera atimu yaikulu yadziko ya Flames yemwe amatumikiraso timuyi Christopher John Banda
Katswiliyu waonedwa ali ndi mtsogoleri wa osewera atimu yaikulu yadziko ya Fulemuzi yemwe amatumikiraso timuyi Khilisitofa Joni Banda
Female
Zikumveka kuti Chipala anapita kukayesa mwai ku UD Songo koma ena mwa akuluakulu atimuyi sakudziwapo kanthu ndipo ndiodabwa chifukwa sakupezeka pa bwalo lazamasewero
Zikumveka kuti Chipala anapita kukayesa mwai ku yudi Songo koma ena mwa akuluakulu atimuyi sakudziwapo kanthu ndipo ndiodabwa chifukwa sakupezeka pa bwalo lazamasewero
Female
pomwe anzake anayamba kupanga zokonzekera. Chaka chatha osewerayu anamwesa zigoli zokwana 9 mu Tnm Super League
pomwe anzake anayamba kupanga zokonzekera. Chaka chatha osewerayu anamwesa zigoli zokwana naini mu Tieni emu supa ligi
Female
Pamene pangodutsa masiku owerengeka osewera wakale pakati watimu ya Nyasa Big Bullets Chimwemwe Idana atasaina kutimu ya Mbeya City ya m'dziko la Tanzania
Pamene pangodutsa masiku owerengeka osewera wakale pakati watimu ya Nyasa Bigi buletsi Chimwemwe Idana atasaina kutimu ya Mbeya site ya m'dziko la Tanzaniya
Female
kwa chaka chimodzi ndi theka, katswiliyu panopa atumikira kae timu ya Silver Strikers kuno ku Malawi pa ngongole kwa miyezi yokwana isanu ndi imodzi
kwa chaka chimodzi ndi theka, katswiliyu panopa atumikira kae timu ya siliva sitilaikazi kuno ku Malawi pa ngongole kwa miyezi yokwana isanu ndi imodzi
Female
Idana waonekera lero ku banja lama central bankers munzinda wa Lilongwe komwe atumikire asanapite kukatumikira kutimu ya Mbeya City transfer window
Idana waonekera lero ku banja lama sentilo bankazi munzinda wa Lilongwe komwe atumikire asanapite kukatumikira kutimu ya Mbeya site thilansifa windo
Female
Idana waonekera lero ku banja lama central bankers munzinda wa Lilongwe komwe atumikire asanapite kukatumikira kutimu ya Mbeya City transfer window ikazasegulidwa
Idana waonekera lero ku banja lama sentilo bankazi munzinda wa Lilongwe komwe atumikire asanapite kukatumikira kutimu ya Mbeya site thilansifa windo ikazatsegulidwa
Female
Timu yomwe yangolowa kumene mu Tnm Super League ku chigawo kwaku m'mwera ya Bangwe All Stars, yalengeza kuti yasaina katswili yemwe amasewera ku Mozambique otchedwa Chimango Kaira
Timu yomwe yangolowa kumene mu Tieni emu supa ligi ku chigawo kwaku m'mwera ya Bangwe ositazi, yalengeza kuti yasaina katswili yemwe amasewera ku Mozambiki otchedwa Chimango Kaira
Female
Kaira yemwe amasewera mutimu ya Vilankulo Fc, wasaina mgwilizano ndi Bangwe All Stars wa zaka ziwili. Osewerayu yemwe amatchuka ndi dzina loti Blackberry
Kaira yemwe amasewera mutimu ya Vilankulo efusi, wasaina mgwilizano ndi Bangwe ositazi wa zaka ziwili. Osewerayu yemwe amatchuka ndi dzina loti Bulakibele
Female
Dzulo timuyi yasainaso osewera awili omwe ndi Innocent Msowoya komaso Bongani Kaipa. Bungwe loyendetsa zisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC)
Dzulo timuyi yasainaso osewera awili omwe ndi Inosenti Msowoya komaso Bongani Kaipa. Bungwe loyendetsa zisankho mdziko muno la Malawi Elekitolo komishoni (MEKI)
Female
lati liyamba mikumano yokonzanso malo atsopano oponyera voti mmadera atsopano a aphungu omwe nyumba ya Malamulo inavomereza mdziko muno
lati liyamba mikumano yokonzanso malo atsopano oponyera voti mmadera atsopano a aphungu omwe nyumba ya Malamulo inavomereza mdziko muno
Female
Mneneli wa bungweli a Sangwani Mwafulirwa ndiwo atsimikiza izi pomwe afotokoza kuti mikumanoyi ichitika kuyambira mwezi uno mpaka mwezi wa March
Mneneli wa bungweli a Sangwani Mwafulirwa ndiwo atsimikiza izi pomwe afotokoza kuti mikumanoyi ichitika kuyambira mwezi uno mpaka mwezi wa Machi
Female
Chaka chatha nyumba ya Malamulo inavomereza kusintha kwa madera a aphungu 193 kufika pa 229
Chaka chatha nyumba ya Malamulo inavomereza kusintha kwa madera a aphungu wani nainte fili kufika pa thuthu naini
Female
Timu ya Karonga United tsopano yalengeza kuti Itenga Kondwani Ikwanga ngati mphunzitsi wamkulu watimuyi
Timu ya Karonga Yunaitedi tsopano yalengeza kuti Itenga Kondwani Ikwanga ngati mphunzitsi wamkulu watimuyi
Female
Timu ya Karonga United tsopano yalengeza kuti yatenga Kondwa Ikwanga ngati mphunzitsi wamkulu watimuyi
Timu ya Karonga yunaitedi tsopano yalengeza kuti yatenga Kondwa Ikwanga ngati mphunzitsi wamkulu watimuyi
Female
Malingana ndi mlembi wamkulu wa Karonga United Ramzy Simwaka, wati mphunzitsiyu yemwe anaphunzitsapo matimu aKatoto United, Super Eagles ndi Jubebox Fc akhala kutimuyi
Malingana ndi mlembi wamkulu wa Karonga yunaitedi lamuze Simwaka, wati mphunzitsiyu yemwe anaphunzitsapo matimu aKatoto yunaitedi, Super igozi ndi Jubebokosi efusi akhala kutimuyi
Female
kwa chaka chonse. Simwaka wanena kuti pakadali pano zonse zofunika zatheka kale ndipo amvana ndi Ikwanga kuti ayambe ntchito yake
kwa chaka chonse. Simwaka wanena kuti pakadali pano zonse zofunika zatheka kale ndipo amvana ndi Ikwanga kuti ayambe ntchito yake
Female
Mphunzitsiyu walowa m'malo mwa Christopher Nyambose yemwe wachoka ndikupita kukakhala mphunzitsi wamkulu watimu ya Tigers
Mphunzitsiyu walowa m'malo mwa khilisitofa Nyambose yemwe wachoka ndikupita kukakhala mphunzitsi wamkulu watimu ya Taigazi
Female
Timu ya Manchester Motor Spares Fc yalengeza kuti osewera awo awili omwe ndi otchinga pagolo yemweso amatumikira timu yachisodzera ya dziko lino ya Malawi under 20
Timu ya Manitchesita mota sipeyazi efusi yalengeza kuti osewera awo awili omwe ndi otchinga pagolo yemweso amatumikira timu yachisodzera ya dziko lino ya Malawi anda twente
Female
Austine Chirambo komaso osewera pakati Gift Sydreck afika m'dziko la Zimbabwe komwe akukayesa mwai kutimu ya Caps United Football Club
Ositini Chirambo komaso osewera pakati Gifiti sidileki afika m'dziko la Zimbabwe komwe akukayesa mwai kutimu ya Kapusi yunaitedi futubo kilabu
Female
Osewera awiliwa afika ku Zimbabwe dzulo lachinai komwe akuyembekezereka kuyamba kuyesa mwai kutimuyi lero lachisanu
Osewera awiliwa afika ku Zimbabwe dzulo lachinai komwe akuyembekezereka kuyamba kuyesa mwai kutimuyi lero lachisanu
Female
Chiwerengero cha osewera ochoka kutimuyi kupita ku Zimbabwe tsopano chafika pa osewera atatu kutsatira kupitaso kwa katswili omwesa zigoli watimuyi
Chiwerengero cha osewera ochoka kutimuyi kupita ku Zimbabwe tsopano chafika pa osewera atatu kutsatira kupitaso kwa katswili omwesa zigoli watimuyi
Female
Emmanuel Banda junior yemwe anapita sabata yatha ndipo akuyesa mwai kutimu ya Dynamos FC. Timu ya Ascent Academy, yauza timu ya Blue Eagles
Imanuwelo Banda juniyo yemwe anapita sabata yatha ndipo akuyesa mwai kutimu ya DynaDainamozi efusi. Timu ya asenti akadame, yauza timu ya Bulu igozi
Female
kuti ipereke ndalama zokwana Five Million Malawi Kwacha kuti igure osewera wao wakutsogolo Christopher Gototo
kuti ipereke ndalama zokwana Faifi miliyoni Malawi Kwacha kuti igure osewera wao wakutsogolo khilisitofa Gototo
Female
Malingana ndi kauniuni wathu, Blue Eagles inalembera kalata timuyi yopempha kuti igure osewera omwesa zigoliyu
Malingana ndi kauniuni wathu, Bulu igozi inalembera kalata timuyi yopempha kuti igure osewera omwesa zigoliyu
Female
pa 6 January 2023 ndipo Ascent inayankha pa 21 January 2023. Muchikalatachi, Ascent yanenaso kuti izapochera nao 10% pa transfer ina
pa sikisi januwale twente twente fili ndipo Asenti inayankha pa twente wani januwale twente twente foli . Muchikalatachi, Asenti yanenaso kuti izapochera nao teni pellesenti pa thilansifa ina
Female
yomwe izachitike pomwe Blue Eagles idzagulise osewerayu ku timu ina. Gototo anakwanisa kumwesa zigoli zisanu mu Tnm Super League ku timu ya Blue Eagles pa nthawi yomwe anabwera ku Nkhwazi
yomwe izachitike pomwe Buli igozi idzagulise osewerayu ku timu ina. Gototo anakwanisa kumwesa zigoli zisanu mu tieniemu supa ligi ku timu ya Bulu igozi pa nthawi yomwe anabwera ku Nkhwazi
Female
zaku area 30 kuchoka kutimu ya Sable Farming. Katswili wakale watimu ya Mighty Mukuru Wanderers Fc Yamikani Chester
zaku eliya fete kuchoka kutimu ya Sebo faming’i. Katswili wakale watimu ya Maite Mukuru Wandeilazi efusi Yamikani Tchesita
Female
tsopano wasaina mgwilizano wa chaka chimodzi ndi timu ya Costa Do Sol ya m'dziko la Mozambique. Chester yemwe sanamvane bwino bwino ndi timu yake Wanderers pofuna kuonjezera mgwilizano okhalira kutimuyi
tsopano wasaina mgwilizano wa chaka chimodzi ndi timu ya Kosita doso ya m'dziko la Mozambiki. Tchesita yemwe sanamvane bwino bwino ndi timu yake wandilazi pofuna kuonjezera mgwilizano okhalira kutimuyi
Female
walengeza kudzera patsamba lake la mchezo la Facebook kuti wasaina timuyi komwe kuliso osewera awili akuno ku Malawi omwe ndi Chikoti Chirwa osewera wakale watimu ya Red Lions
walengeza kudzera patsamba lake la mchezo la Fasibuku kuti wasaina timuyi komwe kuliso osewera awili akuno ku Malawi omwe ndi Chikoti Chirwa osewera wakale watimu ya Redi layonzi
Female
komaso Richard Mbulu osewera wakale watimu ya Mafco. Yamikani Ma Busy Chester analephera kumvana ndi Mighty Mukuru Wanderers Fc nkhani ya ndalama
komaso litchadi Mbulu osewera wakale watimu ya Mafuko. Yamikani Ma bize Tchesita analephera kumvana ndi maite mukulu wandilazi efusi nkhani ya ndalama
Female
yomwe osewera amatenga akasaina contract yomwe muchingerezi imatchulidwa kuti signing on fee. Wachiwiri kwa nduna ya za malo a Deus Gumba
yomwe osewera amatenga akasaina kontilakiti yomwe muchingerezi imatchulidwa kuti sigsaining’i oni fi. Wachiwiri kwa nduna ya za malo a Deusi Gumba
Female
ati malamulo okhudza malo omwe akonzedwanso chaka chatha athandiza kuyendetsa bwino ntchito za malo mdziko muno. A Gumba alakhula izi lachitatu pa nkumano wawo ndi atolankhani amchigawo chapakati
ati malamulo okhudza malo omwe akonzedwanso chaka chatha athandiza kuyendetsa bwino ntchito za malo mdziko muno. A Gumba alakhula izi lachitatu pa nkumano wawo ndi atolankhani amchigawo chapakati
Female
motsogozedwa ndi bungwe la Bwaila Media Club pofuna kuwadziwitsa atolankhani za momwe lamulo latsopano likuyendera
motsogozedwa ndi bungwe la Bwaila midiya kilabu pofuna kuwadziwitsa atolankhani za momwe lamulo latsopano likuyendera
Female
Wachiwiri kwa nduna ya za malo wafotokozanso kufunika kotsata malamulo pa ntchito, wachiwili kwa nduna ya zamalo a Deus Gumba ati malamulo okhuza malo za malo omwe akonzedwaso chaka chatha
Wachiwiri kwa nduna ya za malo wafotokozanso kufunika kotsata malamulo pa ntchito, wachiwili kwa nduna ya zamalo a Deusi Gumba ati malamulo okhuza malo za malo omwe akonzedwaso chaka chatha
Female
Athandiza kuyendetsa bwino ntchito za malo mdziko muno. A Gumba ayankhula izi lachitatu pa mkumano wao ndi atola nkhani amchigawo cha pakati motsogozedwa ndi bungwe la bwaila media club
Athandiza kuyendetsa bwino ntchito za malo mdziko muno. A Gumba ayankhula izi lachitatu pa mkumano wao ndi atola nkhani amchigawo cha pakati motsogozedwa ndi bungwe la bwaila midiya kilabu
Female
pofuna kuwadziwitsa atola nkani za momwe lamuloli likuyendela. Wachiwili kwa nduna ya zamaloyu, wafotokozanso kufunika kotsata malamulo pa ntchito za malo
pofuna kuwadziwitsa atola nkani za momwe lamuloli likuyendela. Wachiwili kwa nduna ya zamaloyu, wafotokozanso kufunika kotsata malamulo pa ntchito za malo
Female
ndi cholinga chopititsa patsogolo chitukuko cha dziko.Ndipo a Horace Nyaka omwe ndi mtsogoleri wa bungwe la atolankhani amchigawo chapakati la Bwaila Media Club
ndi cholinga chopititsa patsogolo chitukuko cha dziko.Ndipo a Holesi Nyaka omwe ndi mtsogoleri wa bungwe la atolankhani amchigawo chapakati la Bwaila mediya kilabu
Female
ati atolankhani akhala akugwiritsa bwino ntchito lamuloli pofikisa mauthenga kwa anthu. Ena mwa malamulowa akupereka mwayi wolembetsa malo omwe anali mmanja mwa anthu ndi mafumu
ati atolankhani akhala akugwiritsa bwino ntchito lamuloli pofikisa mauthenga kwa anthu. Ena mwa malamulowa akupereka mwayi wolembetsa malo omwe anali mmanja mwa anthu ndi mafumu
Female
komanso kupereka mphamvu kwa nduna ya za malo povomereza kapena kukana kupereka chiphaso cha malo. Apolisi m'boma la Thyolo amanga anthu anayi
komanso kupereka mphamvu kwa nduna ya za malo povomereza kapena kukana kupereka chiphaso cha malo. Apolisi m'boma la Thyolo amanga anthu anayi
Female
powaganizira kuti anagwiririra ndi kupha mtsikana wazaka 12 m'bomalo. Wachiwiri kwa wofalitsa nkhani zapolisi m'boma la Thyolo Rabecca Kashoti watsimikizira Ufulu FM online za nkhaniyi
powaganizira kuti anagwiririra ndi kupha mtsikana wazaka twelofu m'bomalo. Wachiwiri kwa wofalitsa nkhani zapolisi m'boma la Thyolo Rabeka Kashoti watsimikizira Ufulu efuemu onilayini za nkhaniyi
Female
A Kashoti ati oganiziridwawa ndi Dan Salijeni wa zaka 26 zakubadwa, Fletcher Selemani zaka 24
A Kashoti ati oganiziridwawa ndi Dani Salijeni wa zaka twente sikisi zakubadwa, Fuletchar Selemani zaka twente folo
Female
Kilinani Kampondeni zaka 26 ndi Andrew Salijeni zaka 29 onsewa a m'bomali
Kilinani Kampondeni zaka twente sikisi ndi Andrew Salijeni zaka twente naini onsewa a m'bomali
Female
Iwo pofotokoza ati pa 17 January chaka chino thupi la mtsikana linapezeka mphepete mwa mtsinje wa Kasembereka
Iwo pofotokoza ati pa seventini januwale chaka chino thupi la mtsikana linapezeka mphepete mwa mtsinje wa Kasembereka
Female
ndipo zotsatira za chipatala zidaonetsa kuti mtsikanayo adagwiriridwa asanaphedwe. A Kashoti ati pakadali pano kafukufuku wa nkhaniyi ali nkati
ndipo zotsatira za chipatala zidaonetsa kuti mtsikanayo adagwiriridwa asanaphedwe. A Kashoti ati pakadali pano kafukufuku wa nkhaniyi ali nkati
Female
Nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo yati amalawi ayembekezere kupitilira kugwa kwa mvula yamphamvu ndi yamabingu mmadera ambiri a dziko lino
Nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo yati amalawi ayembekezere kupitilira kugwa kwa mvula yamphamvu ndi yamabingu mmadera ambiri a dziko lino
Female
kaamba ka namondwe wotchedwa Cheneso yemwe wabuka ku Madagascar ndipo akuyenda kulowa mdziko la Mozambique. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe nthambiyi yatulutsa
kaamba ka namondwe wotchedwa Cheneso yemwe wabuka ku Madagasika ndipo akuyenda kulowa mdziko la Mozambiki. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe nthambiyi yatulutsa
Female
loweruka pa 21 January, 2023 kudzera ku unduna owona zachilengedwe ndi kusintha kwa nyengo
loweruka pa twente wani januwale twente twente fili kudzera ku unduna owona zachilengedwe ndi kusintha kwa nyengo
Female
Kalatayi yati amalawi akhale atcheru ku madzi osefukira omwe adze kaamba ka mvulayi. Chotero, nthambiyi yalangiza anthu onse kuti apewe kuoloka madzi omwe akuthamanga kwambiri
Kalatayi yati amalawi akhale atcheru ku madzi osefukira omwe adze kaamba ka mvulayi. Chotero, nthambiyi yalangiza anthu onse kuti apewe kuoloka madzi omwe akuthamanga kwambiri
Female
kapena omwe atefukira. Timu ya Mighty Mukuru Wanderers Fc lero ikuyembekezereka kusaina katswili osewera mutimu ya dziko lino ya Flames otchinga kumbuyo Lawrence Chaziya
kapena omwe atefukira. Timu ya Maite Mukuru wandilazi efusi lero ikuyembekezereka kusaina katswili osewera mutimu ya dziko lino ya Fulemuzi otchinga kumbuyo Lolensi Chaziya
Female
Malingana ndi zomwe ife tapeza, Chaziya yemwe anasewerapo timu ya Civo Service United asanapite kukasewera ku Jordan timu ya AL Hussein Irbid ali pa ulendo panopa kulowera ku Blantyre
Malingana ndi zomwe ife tapeza, Chaziya yemwe anasewerapo timu ya sivo sevisi yunaitedi asanapite kukasewera ku Jodani timu ya e elo huseni abidi ali pa ulendo panopa kulowera ku Bulantaya
Female
komwe akuyembekezereka kukasaina mgwilizano ndi timu ya Manoma. Osewera yemwe amatchedwa kuti John Stones yu, amafunidwa ndi matimu ena monga Silver Strikers, Nyasa Big Bullets kuno ku Malawi
komwe akuyembekezereka kukasaina mgwilizano ndi timu ya Manoma. Osewera yemwe amatchedwa kuti joni sitonzi yu, amafunidwa ndi matimu ena monga siliva sitilaikazi, Nyasa Bigi Buletsi kuno ku Malawi
Female
komaso matimu ena kunja kwa dziko lino koma Wanderers ndi yomwe yapanga changu kukwanilisa zomwe iye akufuna. Katswiri woyankhulapo pa nkhani zaumoyo George Jobe
komaso matimu ena kunja kwa dziko lino koma Wandilazi ndi yomwe yapanga changu kukwanilisa zomwe iye akufuna. Katswiri woyankhulapo pa nkhani zaumoyo Joji Jobe
Female
wadandaula ndikuchuluka kwa chiwerengero cha anthu omwe akumwalira kaamba ka mlili wa Cholera
wadandaula ndikuchuluka kwa chiwerengero cha anthu omwe akumwalira kaamba ka mlili wa kolela
Female
A Jobe ati kutalikira kwa zipatala zomwe zimathandiza nthenda ya Cholera ndikomwe kukuchulukitsa chiwerengero cha anthu omwalira ndi nthendayi
A Jobe ati kutalikira kwa zipatala zomwe zimathandiza nthenda ya kolela ndikomwe kukuchulukitsa chiwerengero cha anthu omwalira ndi nthendayi
Female
Choyamba, kutalikira kwa zipatala ndikomwe kukuchulukitsa imfazi, wodwala akakhala kuti sanalandire thandizo loyamba kapena kuti First-aid
Choyamba, kutalikira kwa zipatala ndikomwe kukuchulukitsa imfazi, wodwala akakhala kuti sanalandire thandizo loyamba kapena kuti fesiti edi
Female
asanapite kuchipatala komaso chipatala chikatalikira, wodwala otereyo amakhala pa chiopsezo chomwalira atero a Jobe
asanapite kuchipatala komaso chipatala chikatalikira, wodwala otereyo amakhala pa chiopsezo chomwalira atero a Jobe
Female
A Jobe awonjezeranso kuti zikhulupiliro zoti munthu akumamwalira akapititsidwa ku chipatala ndizomwe zikuchulutsa chiwerengerochi pamene anthu 852 ndiomwe amwalira chiyambireni cha mlili wa Cholera
A Jobe awonjezeranso kuti zikhulupiliro zoti munthu akumamwalira akapititsidwa ku chipatala ndizomwe zikuchulutsa chiwerengerochi pamene anthu eiti handede andi fifite thu ndiomwe amwalira chiyambireni cha mlili wa kolela
Female
Timu ya Kamuzu Barracks Fc yalengeza kuti yalora osewera atatu omwe ndi Mustafa Maulana komaso Blessings Chimbaza omwe ndi otchinga kumbuyo komaso m'modzi omwesa zigoli otchedwa Temwa Msowoya
Timu ya Kamuzu Balakisi efusi yalengeza kuti yalora osewera atatu omwe ndi Musitafa Maulana komaso Blesing’izi Chimbaza omwe ndi otchinga kumbuyo komaso m'modzi omwesa zigoli otchedwa Temwa Msowoya
Female
kuti apite ku timu iliyonse yomwe angafune. Timuyi yalengeza izi kudzera mu Kalata yomwe yatulutsa posachedwapa
kuti apite ku timu iliyonse yomwe angafune. Timuyi yalengeza izi kudzera mu Kalata yomwe yatulutsa posachedwapa
Female
Osewera awili omwe ndi Blessings Chimbaza komaso Temwa Msowoya anabwera kutimuyi atatengedwa ku Kamuzu Barracks Reserve pomwe Mustafa Maulana anachokera kutimu ya Ekwendeni Hammers
Osewera awili omwe ndi Blesing’izi Chimbaza komaso Temwa Msowoya anabwera kutimuyi atatengedwa ku Kamuzu BarBalakisi lizevu pomwe Musitafa Maulana anachokera kutimu ya Ekwendeni Hamazi
Female
Nsika wa kwa Manje madzi kusefukira mu Nsewu. Aka koyamba nsewuwu chimangidwireni kamba kosowa ngalande za zopatutsira madziwa
Nsika wa kwa Manje madzi kusefukira mu Nsewu. Aka koyamba nsewuwu chimangidwireni kamba kosowa ngalande za zopatutsira madziwa
Female