audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
Mwambo omwe wayamba loweluka pa 3 February ndipo ukuyembekezeka kutha pa 7 February 2024 | Mwambo omwe wayamba loweluka pa fili febuluwale ndipo ukuyembekezeka kutha pa seveni febuluwale twente twente folo | Female | |
Mmodzi mwa amene akudzapikisana nao pa zisankho za phungu wa nyumba yamalamulo mdera la Machinga south East constituency Alexander Synoden | Mmodzi mwa amene akudzapikisana nao pa zisankho za phungu wa nyumba yamalamulo mdera la Machinga saufi isiti konsitichuwense alekizanda sinodeni | Female | |
watsimikizira anthu a delali kuti ndizotheka kukhala ndi dela lotukuka ngati mmene alili Madera ena a dziko lino | watsimikizira anthu a delali kuti ndizotheka kukhala ndi dela lotukuka ngati mmene alili Madera ena a dziko lino | Female | |
Iye wati izi zingachitike pomwe anthu ataika chidwi pantchito zachitukuko komanso kukhala ndi atsogoleli okonda delali | Iye wati izi zingachitike pomwe anthu ataika chidwi pantchito zachitukuko komanso kukhala ndi atsogoleli okonda delali | Female | |
Alexander Synoden amene anati iye ndi mbadwa ya delali ndipo akudziwa bwino zofuna za anthu a Machinga South East constituency amalankhula izi Lamulungu pa 28 January 2024 ndi Angaliba | Alekizanda sinodeni amene anati iye ndi mbadwa ya delali ndipo akudziwa bwino zofuna za anthu a Machinga saufi isiti consitichuwense amalankhula izi Lamulungu pa twente eiti januwale twente twente folo ndi Angaliba | Female | |
pomwe amalongosola za masomphenya ake ozatenga mbali pa zisankhozi.Iye anati anthu a ku Machinga South East avutika kokwanira ndipo pakufunika kuchitapo kanthu powabweretsera zofuna zao | pomwe amalongosola za masomphenya ake ozatenga mbali pa zisankhozi.Iye anati anthu a ku Machinga saufi isiti avutika kokwanira ndipo pakufunika kuchitapo kanthu powabweretsera zofuna zao | Female | |
Synoden ananena kuti akudzapikisana nao pa mpando wa phungu wa nyumba yamalamulo ngati oyima payekha | Sinodeno ananena kuti akudzapikisana nao pa mpando wa phungu wa nyumba yamalamulo ngati oyima payekha | Female | |
Ndidzaimira ngati wa independent pakuti ndikuimira anthu onse a derali osati a chipani chimodzi.Zosankhana potsogoza ndale ndi zomwe zikuononga dzikoli.Anatero Synoden | Ndidzaimira ngati wa independent pakuti ndikuimira anthu onse a derali osati a chipani chimodzi. Zosankhana potsogoza ndale ndi zomwe zikuononga dzikoli.Anatero Sinodeni | Female | |
Mmau ake omaliza anapempha mafumu kuti agwirane manja ndicholinga chofuna kupanga delali kukhala lotukuka pa ntchito zamalonda | Mmau ake omaliza anapempha mafumu kuti agwirane manja ndicholinga chofuna kupanga delali kukhala lotukuka pa ntchito zamalonda | Female | |
umoyo wabwino, Mayendedwe osavuta, Magetsi paliponse, School zabwino,Chitetezo ndi kusasowa chakudya zomwe anati izi ndizomwe anthu akuzisaukira | umoyo wabwino, Mayendedwe osavuta, Magetsi paliponse, Sukulu zabwino,Chitetezo ndi kusasowa chakudya zomwe anati izi ndizomwe anthu akuzisaukira | Female | |
Polankhula mwapadera mmodzi mwa mzika ya delali Hanif Maloya anati ndiokodwa kuona kuti achinyamata akuona mwa chidwi mavuto a delali | Polankhula mwapadera mmodzi mwa mzika ya delali Hanifi Maloya anati ndiokodwa kuona kuti achinyamata akuona mwa chidwi mavuto a delali | Female | |
Chomcho Maloya anamema anthu kuti atsatile a Synoden ponena kuti ali ndi mfundo zolondeka zomwe zingatukule Machinga South East constituency | Chomcho Maloya anamema anthu kuti atsatile a Sinodeni ponena kuti ali ndi mfundo zolondeka zomwe zingatukule Machinga saufi isiti konsitichuwense | Female | |
Mkulu wa Malawi Communication Regulatory Authority (MACRA), Daud Suleman wati ntchito yopeleka nambala zatsopano ku nyumba zofalitsa mawu yayenda bwino | Mkulu wa Malawi komyunikeshoni legyuletale ofolite (MAKIRA), Daudi Sulemani wati ntchito yopeleka nambala zatsopano ku nyumba zofalitsa mawu yayenda bwino | Female | |
Iwo ayankhula izi lachiwiri muzinda wa Lilongwe pamsonkhano wa atolankhani. A Suleman anati ntchitoyi yayenda bwino chifukwa anagwira limodzi ndi anthu ogwira ntchito kunyumba zofalitsa nkhani | Iwo ayankhula izi lachiwiri muzinda wa Lilongwe pamsonkhano wa atolankhani. A Sulemani anati ntchitoyi yayenda bwino chifukwa anagwira limodzi ndi anthu ogwira ntchito kunyumba zofalitsa nkhani | Female | |
Izi zipeleka danga loti nyumba zina zofalitsa nkhani m'dziko muno zibwere ndipo anthu apeza ntchito komaso kukhala ndi mwayi wosankha wayilesi yakumtima kwawo | Izi zipeleka danga loti nyumba zina zofalitsa nkhani m'dziko muno zibwere ndipo anthu apeza ntchito komaso kukhala ndi mwayi wosankha wayilesi yakumtima kwawo | Female | |
Pali pano bungwe la MACRA labweretsa makina awiri omwe athandize ntchito za bungweli ena mwa makinawo athandize kuthetsa mchitidwe woberana ndalama mu foni | Pali pano bungwe la MAKIRA labweretsa makina awiri omwe athandize ntchito za bungweli ena mwa makinawo athandize kuthetsa mchitidwe woberana ndalama mu foni | Female | |
Pakadali pano makinawa alumikizidwa kale ku ma network onse m'dziko muno. Podzafika pa 1 April makina awiri onsewa akhala atayamba kugwira ntchito m'dziko muno, anatero a Suleman | Pakadali pano makinawa alumikizidwa kale ku ma netiweki onse m'dziko muno. Podzafika pa wani epulo makina awiri onsewa akhala atayamba kugwira ntchito m'dziko muno, anatero a Sulemani | Female | |
Media Council of Malawi (MCM) anakonza maphunziro Kwa atolankhani okhudzana ndi momwe angalembele nkhani komanso ukadaulo wa momwe angapezele uthenga ofunikila mosavuta | MediaMidiya khanso ofu Malawi (Emusiemu) anakonza maphunziro Kwa atolankhani okhudzana ndi momwe angalembele nkhani komanso ukadaulo wa momwe angapezele uthenga ofunikila mosavuta | Female | |
Polankhula executive director wa Media Council of Malawi a Moses Kaufa pazochitikazo zomwe zinachitika pa 23 January 2024 | Polankhula ekizekitivi dailekita wa midiya khanso ofu Malawi a Mozesi Kaufa pazochitikazo zomwe zinachitika pa twente fili januwale twente twente folo | Female | |
ku Malawi Sun Hotel mu mzinda wa Blantyre anamema atolankhani kugwiritsantchito akadaulo pantchito yao | ku Malawi Sani Hotelo mu mzinda wa Bulantaya anamema atolankhani kugwiritsantchito akadaulo pantchito yao | Female | |
A Kaufa ati atolankhani akuyenera kudziwa bwino momwe angalembele nkhani zokhuzana ndi zinthu zina monga nkhani zokhudzana ndi kugwililidwa mcholinga chofuna kuteteza ufulu wa olakwilidwawo | A Kaufa ati atolankhani akuyenera kudziwa bwino momwe angalembele nkhani zokhuzana ndi zinthu zina monga nkhani zokhudzana ndi kugwililidwa mcholinga chofuna kuteteza ufulu wa olakwilidwawo | Female | |
Ndipo anapitiliza mkunena kuti Iwo akufunitsisa kuti awone atolankhani akulemba nkhani zawo mopanda kuwonjezela kapena kuchosela chilichonse | Ndipo anapitiliza mkunena kuti Iwo akufunitsisa kuti awone atolankhani akulemba nkhani zawo mopanda kuwonjezela kapena kuchosela chilichonse | Female | |
Ngati njira imodzi yopanga atolankhani kukhala odzidalila pachuma gulu la atolankhani a mchigao chakummwela kwa dziko lino lotchedwa Southern Region Press Club | Ngati njira imodzi yopanga atolankhani kukhala odzidalila pachuma gulu la atolankhani a mchigao chakummwela kwa dziko lino lotchedwa Sauveni lijoni pulesi kilabu | Female | |
lagula malo omwe cholinga chake ndikuchitapo ulimi wa ziweto. Malowa agulidwa mu mzinda wa Lilongwe mmudzi mwa Whayo mfumu yaikulu Kapeni | lagula malo omwe cholinga chake ndikuchitapo ulimi wa ziweto. Malowa agulidwa mu mzinda wa Lilongwe mmudzi mwa Whayo mfumu yaikulu Kapeni | Female | |
Polankhula ndi Angaliba Ronard Amos amene ndi Mkhalapampando wa gululi wati Malowa ndi okwana hectare imodzi ndipo Pali ganizo lakuti pamalopa paziwetedwa ziweto | Polankhula ndi Angaliba Ronadzi Amosi amene ndi Mkhalapampando wa gululi wati Malowa ndi okwana hekita imodzi ndipo Pali ganizo lakuti pamalopa paziwetedwa ziweto | Female | |
zomwe phindu lake lipindulile mamembala a gululi. Iye anati apeza kale akadaulo omwe aphunzitse bwino atolankhani momwe angapangire ulimiwu kuti ukhale wa phindu | zomwe phindu lake lipindulile mamembala a gululi. Iye anati apeza kale akadaulo omwe aphunzitse bwino atolankhani momwe angapangire ulimiwu kuti ukhale wa phindu | Female | |
Komabe iye anapempha akufuna kwabwino kuti athandize gululi pofuna kukwaniritsa masomphenya awo. Gululi lomwe padakali pano lili ndi mamembala opitilila one hundred | Komabe iye anapempha akufuna kwabwino kuti athandize gululi pofuna kukwaniritsa masomphenya awo. Gululi lomwe padakali pano lili ndi mamembala opitilila wani handiledi | Female | |
linakhanzikitsidwa chaka chatha mwezi wa December. Unduna wa zaumoyo ndi thandizo lochokela ku Momentum Tiyeni Project anakonza mkumano ndi atolankhani | linakhanzikitsidwa chaka chatha mwezi wa Disemba. Unduna wa zaumoyo ndi thandizo lochokela ku Momentamu Tiyeni Pulojekiti anakonza mkumano ndi atolankhani | Female | |
pofuna kuwunikira mmene angalembere nkhani zokhudza zaumoyo. Mkumanowu unachitika lolemba ku Mount Soche Hotel mu nzinda wa Blantyre | pofuna kuwunikira mmene angalembere nkhani zokhudza zaumoyo. Mkumanowu unachitika lolemba ku Maunti soche Hotelo mu nzinda wa Bulantaya | Female | |
Poyankhula ndi Angaliba Dr Owen Chimkwaza omwe ndi wachiwiri kwa mkulu wa Reproductive Health anati project yao yothandiza ana ndi amayi ikuyenda bwino | Poyankhula ndi Angaliba Dokota Oweni Chimkwaza omwe ndi wachiwiri kwa mkulu wa lipulodakitivi hefe anati pulojekiti yao yothandiza ana ndi amayi ikuyenda bwino | Female | |
Dr Chinkwaza anati amayi mdziko muno akutaya miyoyo panthawi yobereka komanso atsikana akubeleka asanankhwime | Dokota Chinkwaza anati amayi mdziko muno akutaya miyoyo panthawi yobereka komanso atsikana akubeleka asanankhwime | Female | |
Iwo anatsindika kunena kuti akufunitsitsa kuti pofika chaka cha 2030 azakhale atathana ndi mavutowa | Iwo anatsindika kunena kuti akufunitsitsa kuti pofika chaka cha twente fete azakhale atathana ndi mavutowa | Female | |
Kumbali yawo a John Sande omwe ndi ochokela ku Malawi Malaria Program anati kumbali ya nthenda ya malungo mukupezekabe chiwerengero chokwera cha anthu maka amayi | Kumbali yawo a Joni Sande omwe ndi ochokela ku Malawi Maleliya pulogalamu anati kumbali ya nthenda ya malungo mukupezekabe chiwerengero chokwera cha anthu maka amayi | Female | |
Koma a Sande ati posachedwapa akhale akugawa ma Ukonde ozitetezera ku Udzudzu m'maboma onse adziko muno | Koma a Sande ati posachedwapa akhale akugawa ma Ukonde ozitetezera ku Udzudzu m'maboma onse adziko muno | Female | |
Athu aku kasungu Khawa yakula tsopano pomwe Madzi akhala pafupifupi masiku anai asanatuuluke | Athu aku kasungu Khawa yakula tsopano pomwe Madzi akhala pafupifupi masiku anai asanatuuluke | Female | |
Modzi mwa athu okhudzidwa a Brian Sephas ati madzi omwe iwo akugwilitsa ntchito ndioipa zimene zikuika miyoyo yawo pa chiopsezo chodwala matenda a cholera | Modzi mwa athu okhudzidwa a Bulayani Sefasi ati madzi omwe iwo akugwilitsa ntchito ndioipa zimene zikuika miyoyo yawo pa chiopsezo chodwala matenda a kolela | Female | |
Izi zikuchitika pomwe bungwe logawa madzi la central region water board litalengezetsa kut madzi akhala akuvuta madera ozungulira town ya Kasungu | Izi zikuchitika pomwe bungwe logawa madzi la sentilo lijoni wota bodi litalengezetsa kut madzi akhala akuvuta madera ozungulira tauni ya Kasungu | Female | |
Bwalo la milandu ku Mangochi kudzera mwa senior resident Magistrate Muhammad Maxwell Chande laimitsa mlandu wa Bon Kalindo amene ndi mtsogoleri wa gulu lotchedwa Malawi First | Bwalo la milandu ku Mangochi kudzera mwa siniyo lezidenti majesitileti muhamadi makisiwelo Chande laimitsa mlandu wa Boni Kalindo amene ndi mtsogoleri wa gulu lotchedwa Malawi Fesiti | Female | |
kufikira pa 9 February 2024 poyembekezera makalata a maumboni ochokera ku mbali zonse zokhudzidwa. A Kalindo amene padakali pano ali pabelo akuyankha mulandu woyambitsa chisokonezo | kufikira pa naini febuluwale twente twente folo poyembekezera makalata a maumboni ochokera ku mbali zonse zokhudzidwa. A Kalindo amene padakali pano ali pabelo akuyankha mulandu woyambitsa chisokonezo | Female | |
kudzera pa zionetsero zomwe zinachtika pa 30 November 2023 zosagwirizana ndi kutsika mphanvu kwa ndalama ya kwacha | kudzera pa zionetsero zomwe zinachtika pa fete novemba twente twente fili zosagwirizana ndi kutsika mphanvu kwa ndalama ya kwacha | Female | |
Mboni za boma lelo zaperekera umboni ndipo atsindikiza kuti chisokonezo chinabwera kamba ka zionetselozi | Mboni za boma lelo zaperekera umboni ndipo atsindikiza kuti chisokonezo chinabwera kamba ka zionetselozi | Female | |
komabe mbonizo sizinalankhule mulunjika ngati anaona kapena kumva a Kalindo akumeneza anthu kuti achite ziwawa | komabe mbonizo sizinalankhule mulunjika ngati anaona kapena kumva a Kalindo akumeneza anthu kuti achite ziwawa | Female | |
Bwaloli likangolandila makalatao likuyembekezeka kudzagamula ngati Pali mlandu kapena ai. Bungwe lowona mayenso m'dziko muno la Malawi National Examinations Board (MANEB) | Bwaloli likangolandila makalatao likuyembekezeka kudzagamula ngati Pali mlandu kapena ai. Bungwe lowona mayenso m'dziko muno la Malawi neshono ekizamineshoni bodi (MANEBU) | Female | |
lowonjezera nthawi yolipilira Mayenso a Primary School Leaving Certificate, Junior Certificate of Education ndi Malawi School Certificate of Education kuchoka pa 31 December 2023 | lowonjezera nthawi yolipilira Mayenso a Pulaimale Sukulu Living’i Satifiketi, Juniyo satifiketi ofu ejukeshoni ndi Malawi sukulu satifiketi ofu ejukeshoni kuchoka pa fete wani disemba twente twente fili | Female | |
kufika usiku wa12 January 2024. Izi ndi Malinga ndi kalata yomwe bungweli yatulutsa lachiwiri pa 9January 2024 yomwe yasainidwa ndi mkulu wa bungweli Professor Dorothy Nampota | kufika usiku wa thwelofu januwale twente twente folo. Izi ndi Malinga ndi kalata yomwe bungweli yatulutsa lachiwiri pa naini januwale twente twente folo yomwe yasainidwa ndi mkulu wa bungweli pulofesa dolofe Nampota | Female | |
Kuwonjezeraku kuthandiza ophunzira omwe analephera kulipira mayeso mu nthawi yathayi. Bungwe la MANEB lalimbikitsa ophunzira, makolo ndi ena onse | Kuwonjezeraku kuthandiza ophunzira omwe analephera kulipira mayeso mu nthawi yathayi. Bungwe la MANEBU lalimbikitsa ophunzira, makolo ndi ena onse | Female | |
kugwiritsa ntchito njira zovomelezeka zolipira mayeso monga TNM Mpamba komaso ma bank. Aphungu a nyumba ya malamulo akuyembekezeka kuyamba zokambirana zawo za chinayi | kugwiritsa ntchito njira zovomelezeka zolipira mayeso monga Tieniemu Mpamba komaso ma banki. Aphungu a nyumba ya malamulo akuyembekezeka kuyamba zokambirana zawo za chinayi | Female | |
mu mkumano wa nyumba ya malamulo wanambala 50 pa 9 February 2024. Malingana ndi sipikala wa nyumbayi Catherine Gotani Hara, wati mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera | mu mkumano wa nyumba ya malamulo wanambala fifite pa naini febuluwale twente twente folo. Malingana ndi sipikala wa nyumbayi kafelini Gotani Hara, wati mtsogoleri wa dziko lino Dokota Lazalazi Chakwera | Female | |
akuyembekezeka kudzatsegulira mkumanowu nthawi ya 10 koloko m'mawa. Mwazina aphungu m'nyumbayi akuyembekezeka kudzakambirana ndondomeko ya zachuma | akuyembekezeka kudzatsegulira mkumanowu nthawi ya teni koloko m'mawa. Mwazina aphungu m'nyumbayi akuyembekezeka kudzakambirana ndondomeko ya zachuma | Female | |
ya chaka cha 2024 mpaka 2025. Panakali pano, unduna wa zachuma uli mkati mofunsa maganizo a magulu osiyanasiyana | ya chaka cha twente twente folo mpaka twente twente faifi. Panakali pano, unduna wa zachuma uli mkati mofunsa maganizo a magulu osiyanasiyana | Female | |
pa zomwe akufuna kuti zikhale mu ndondomeko ya za chuma yomwe aphunguwa akhale akukambirana posachedwapa. Zokambiranazi zikuyembekezeka kudzatha pa 5 April 2024 | pa zomwe akufuna kuti zikhale mu ndondomeko ya za chuma yomwe aphunguwa akhale akukambirana posachedwapa. Zokambiranazi zikuyembekezeka kudzatha pa 5faifi epulo twente twente folo | Female | |
Yemwe akufuna kudzaimira ngati phungu wa nyumba ya Malamulo mu dera la Masintha Constituency a Joseph Chasweka wati, iye monga mzika | Yemwe akufuna kudzaimira ngati phungu wa nyumba ya Malamulo mu dera la Masintha konsitichuwense a jozefe Chasweka wati, iye monga mzika | Female | |
akufunitsitsa kutuluka dera la Masintha Constituency zomwe anthu ambiri ozungulira derali amupepha | akufunitsitsa kutuluka dera la Masintha konsitichuwense zomwe anthu ambiri ozungulira derali amupepha | Female | |
Achasweka amayankhula izi pakutha pa masewero womwe anakhazikitsa ngati njira imodzi yofuna kuwazindikiritsa anthu za chidwi chawo chofuna kuimira ngati phungu wa nyumba ya Malamulo | Achasweka amayankhula izi pakutha pa masewero womwe anakhazikitsa ngati njira imodzi yofuna kuwazindikiritsa anthu za chidwi chawo chofuna kuimira ngati phungu wa nyumba ya Malamulo | Female | |
Masewero womwe analipo pakati pa ma team a Condos komanso Green Boys adera la Kawale 1 ndi 2, omwe akatswiri ake ndi team ya Condos yomwe inapambana ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi | Masewero womwe analipo pakati pa ma timu a kondozi komanso gilini boyizi adera la Kawale wani ndi thu, omwe akatswiri ake ndi team ya kondozi yomwe inapambana ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi | Female | |
Mabonanza omwe anakhazikitsa dera la Chilinde, Kawale ndipo akuyembekezanso kukamaliza ndi dera la Mchesi ndi Biwi lamulungu likudzali | Mabonanza omwe anakhazikitsa dera la Chilinde, Kawale ndipo akuyembekezanso kukamaliza ndi dera la Mchesi ndi Biwi lamulungu likudzali | Female | |
Dera lililonse akuika ndalama zokwana 1.4 million, zomwe madera onsewa kwakwana 4.5 million | Dera lililonse akuika ndalama zokwana wani pointi folo miliyoni, zomwe madera onsewa kwakwana fo pointi faifi miliyoni | Female | |
Pamwambowo anaitana a Patrick Macheso ngati mlendo wolemekezeka ndipo iye anati masewera ngati awa amaoneka ngati wopanda pake koma ndi masewera omwe amafukula luso achinyamata ambiri | Pamwambowo anaitana a Patiliki Macheso ngati mlendo wolemekezeka ndipo iye anati masewera ngati awa amaoneka ngati wopanda pake koma ndi masewera omwe amafukula luso achinyamata ambiri | Female | |
ndipo analimbikitsa aphungu a nyumba ya Malamulo kuti adziganizilanso nkhani za masewero komanso kukonza mabwalo kuti adzikhala abwino | ndipo analimbikitsa aphungu a nyumba ya Malamulo kuti adziganizilanso nkhani za masewero komanso kukonza mabwalo kuti adzikhala abwino | Female | |
Joseph Chasweka ndi mmodzi mwa anthu azamalonda mu dera la Chilinde yemwe ndi mwini wake wa Chipatala cha 24 hours | Joseph Chasweka ndi mmodzi mwa anthu azamalonda mu dera la Chilinde yemwe ndi mwini wake wa Chipatala cha twente folo awazi | Female | |
Apolice ku Monkey Bay alangiza anthu kuti apewe kukhala malo amene amapezeka Ng'ona. Mawuwa adza kutsatira munthu wina amene wagwidwa ndi Ng'ona ndipo mpaka pano sakuoneka | Apolice ku Monkibe alangiza anthu kuti apewe kukhala malo amene amapezeka Ng'ona. Mawuwa adza kutsatira munthu wina amene wagwidwa ndi Ng'ona ndipo mpaka pano sakuoneka | Female | |
Mneneri wa apolice ya Monkey Bay Sergeant Alice Sichali wati munthuyo dzina lake ndi Kazuwa Ali | Mneneri wa apolice ya Monkibe sajenti alisi Sichali wati munthuyo dzina lake ndi Kazuwa Ali | Female | |
Chilombochi chinamungwira pomwe amkakapanga ntchito ya usodzi m'banda kucha wa lachiwiri pa 9 January 2024. Asodzi ena anayesetsa kumupulumutsa komabe sizinatheke | Chilombochi chinamungwira pomwe amkakapanga ntchito ya usodzi m’banda kucha wa lachiwiri pa naini januwale twente twente folo. Asodzi ena anayesetsa kumupulumutsa komabe sizinatheke | Female | |
Padakali pano apolice akupitiliza kuyang'ana. FCB Nyasa Bullets yakhala akatswiri a chikho cha Airtel top 8 itangogonjetsa timu ya Mafco ndi zigoli ziwiri Kwa chimodzi | Padakali pano apolisi akupitiliza kuyang'ana. Efisibi nyasa buletsi yakhala akatswiri a chikho cha eyatelo topu eiti itangogonjetsa timu ya Mafuko ndi zigoli ziwiri Kwa chimodzi | Female | |
FCB Nyasa Bullets inapeza zigoli kudzera mwa Lanjesi Nkhoma. Pomwe timu ya Mafco inapeza chigoli chomwe Nickson Nyasulu anadzigolera mu mphundi 35 za chigawo choyamba chamasewerowa | Efusibi Nyasa Buletsi inapeza zigoli kudzera mwa Lanjesi Nkhoma. Pomwe timu ya Mafuko inapeza chigoli chomwe Nikisoni Nyasulu anadzigolera mu mphundi fete faifi za chigawo choyamba chamasewerowa | Female | |
Kutsatila kuchotsedwa kwa pempho lofuna kumva madando awo ku bwalo la milandu Mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma a Kondwani Nankhumwa | Kutsatila kuchotsedwa kwa pempho lofuna kumva madando awo ku bwalo la milandu Mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma a Kondwani Nankhumwa | Female | |
omwenso ndi mmodzi mwa omwe akufuna kupikisana nawo pa pulezidenti ngati prezidenti wa chipani cha DPP wati akufunsira uphungu pa za tsogolo lawo pandale | omwenso ndi mmodzi mwa omwe akufuna kupikisana nawo pa pulezidenti ngati prezidenti wa chipani cha Dipipi wati akufunsira uphungu pa za tsogolo lawo pandale | Female | |
ndipo ati posachedwapa alengeza za tsogololi. Izi zadza potsatira chigamulo cha bwalo la Apilo chomwe chathetsa mulandu | ndipo ati posachedwapa alengeza za tsogololi. Izi zadza potsatira chigamulo cha bwalo la Apilo chomwe chathetsa mulandu | Female | |
omwe a Nankhumwa ndi atsogoleri ena anasumila Professor Peter Mutharika powasintha mmaudindo awo. Malingana ndi kalata imene atulutsa yomwe Angaliba yaona iwo ati polemekeza ma bwalo a milandu | omwe a Nankhumwa ndi atsogoleri ena anasumila pulofesa pita Mutharika powasintha mmaudindo awo. Malingana ndi kalata imene atulutsa yomwe Angaliba yaona iwo ati polemekeza ma bwalo a milandu | Female | |
akuvomereza chigamulocho, ngakhale kuli kovuta kugwirizana ndi zotsatira zake. Mtsogoleri wa chipanichi Proffessor Peter Munthalika anasintha ena mwa Maudindo chipanichi | akuvomereza chigamulocho, ngakhale kuli kovuta kugwirizana ndi zotsatira zake. Mtsogoleri wa chipanichi Pulofesa Pita Munthalika anasintha ena mwa Maudindo chipanichi | Female | |
zomwe sizinakondweretse a Nankhumwa ndi gulu lao.Iwo adapatsidwa udindo okhala mlangizi wa a Munthalika. Abusa ndithandizeni ndikusoweka thandizo | zomwe sizinakondweretse a Nankhumwa ndi gulu lao.Iwo adapatsidwa udindo okhala mlangizi wa a Munthalika. Abusa ndithandizeni ndikusoweka thandizo | Female | |
munthune ndikapeza mlongo omanga naye banja moyo wanga umayamba kukonda azimzake kuposa mlongoyo. Mapeto ake chibwenzi chija chimapezeka chatha ndipo ndatengana ndi mzake uja | munthune ndikapeza mlongo omanga naye banja moyo wanga umayamba kukonda azimzake kuposa mlongoyo. Mapeto ake chibwenzi chija chimapezeka chatha ndipo ndatengana ndi mzake uja | Female | |
Koma ndi mzake uja sichimakhalitsanso. Nditani abusa, munthune ndufuna kukwatila mutidalitse chaka chino. Iyayi nenani chilungamo Azibambo | Koma ndi mzake uja sichimakhalitsanso. Nditani abusa, munthune ndufuna kukwatila mutidalitse chaka chino. Iyayi nenani chilungamo Azibambo | Female | |
atakhala mkazi wanu wayamba kuyimba nkukapanga izi pa golf club ndi Praise Umali muyilola. Nanga inu azimayi mwamuna wanu oyimba akapange izi pa Gymkana ndi Tuno muyilola | atakhala mkazi wanu wayamba kuyimba nkukapanga izi pa gofu kilabu ndi Pulezi Umali muyilola. Nanga inu azimayi mwamuna wanu oyimba akapange izi pa Jinkana ndi Tuno muyilola | Female | |
Inu Usher ndi Alicia akuoneka osangalala kuposa masiku onse. Inu amvana kukoma awa. Kuchita kusangalatsa | Inu Asha ndi Alisha akuoneka osangalala kuposa masiku onse. Inu amvana kukoma awa. Kuchita kusangalatsa | Female | |
Tsiku lina dzaka zam'mbuyomo makolo a anawa adangochoka pakhomo ndipo sadabwerenso mpaka lero. Kodi adapita kuti | Tsiku lina dzaka zam'mbuyomo makolo a anawa adangochoka pakhomo ndipo sadabwerenso mpaka lero. Kodi adapita kuti | Female | |
Nanga anawa chakudya, rent ndi zina amazipeza bwanji. Mwana wooneka wamkuluyu, Maria, ali ndi dzaka 15 | Nanga anawa chakudya, renti ndi zina amazipeza bwanji. Mwana wooneka wamkuluyu, Mariya, ali ndi dzaka fifitini | Female | |
ndipo amagwira maganyu otunga madzi ndi kuchapa m'makomo kuti azilera azibale ake tikhala akucheza ndi Maria ndi azibale ake pa program ya The Citizen | ndipo amagwira maganyu otunga madzi ndi kuchapa m'makomo kuti azilera azibale ake tikhala akucheza ndi Mariya ndi azibale ake pa pulogalamu ya ve sitizeni | Female | |
ili ndi phunziro kuti anthu azijama yawo ngat sakwanitsa azijama ya amawo ndabambwawo. Ku Malawi kuno china chimene timasaukira kwambiri nd kujama ya anthu ena kusiya yathu | ili ndi phunziro kuti anthu azijama yawo ngat sakwanitsa azijama ya amawo ndabambwawo. Ku Malawi kuno china chimene timasaukira kwambiri nd kujama ya anthu ena kusiya yathu | Female | |
Kwatuluka chi kalata kuchoka ku SMAM chopita kwa anyamata awiri ena amene adatenga akazi awo nkukawafunsilila kunja kwa dziko wina ku Dubai, wina ku Newyork | Kwatuluka chi kalata kuchoka ku Simamu chopita kwa anyamata awiri ena amene adatenga akazi awo nkukawafunsilila kunja kwa dziko wina ku Dubai, wina ku Nyuyoko | Female | |
Chikalatachi chakupezani kale. Ngati sichinafike chili kuma comment ku Oyimba ena akulu akulu collabo yawo yoyamba ayimbila mkazi wa Tonderai, Tahera. Ndipo ajambula video yatuluka | Chikalatachi chakupezani kale. Ngati sichinafike chili kuma komenti ku Oyimba ena akulu akulu kolabo yawo yoyamba ayimbila mkazi wa Tonderai, Tahera. Ndipo ajambula vidiyo yatuluka | Female | |
Yehova adzatsekula kumwamba kumene amasungirako chuma chake, kutumiza mvula mʼdziko lanu pa nthawi yake ndi kudalitsa ntchito yonse ya manja anu | Yehova adzatsekula kumwamba kumene amasungirako chuma chake, kutumiza mvula mʼdziko lanu pa nthawi yake ndi kudalitsa ntchito yonse ya manja anu | Female | |
Mudzakongoza mitundu yambiri koma inu simudzakongola kwa aliyense Zimatele maluzi akakuthibula koma anthu ena amene umafanana nawo | Mudzakongoza mitundu yambiri koma inu simudzakongola kwa aliyense Zimatele maluzi akakuthibula koma anthu ena amene umafanana nawo | Female | |
Chenjelani ndi maubwenzi a pamasamba a mchezo_mangochi police. Apolisi m'boma la Mangochi achenjeza anthu kuti apewe kutengeka ndi anthu osadziwika maka pa masamba a mchezo poopa kuberedwa | Chenjelani ndi maubwenzi a pamasamba a mchezo_mangochi polisi. Apolisi m'boma la Mangochi achenjeza anthu kuti apewe kutengeka ndi anthu osadziwika maka pa masamba a mchezo poopa kuberedwa | Female | |
Chenjezoli lomwe laperekedwa ndi mneneri wa polisi ya Mangochi inspector Amina Tepani Daudi ladza kutsatila kumangwidwa kwa mnyamata wina amene wakhala akubera anthu mu mdzina la chikondi | Chenjezoli lomwe laperekedwa ndi mneneri wa polisi ya Mangochi insipekita Amina Tepani Daudi ladza kutsatila kumangwidwa kwa mnyamata wina amene wakhala akubera anthu mu mdzina la chikondi | Female | |
Junior M'bwana wa zaka 24 zakubadwa amumanga pomuganizira kuti wakhala akubera akazi powanamiza zachikondi kudzera pa Facebook | Juniyo M'bwana wa zaka twente folo zakubadwa amumanga pomuganizira kuti wakhala akubera akazi powanamiza zachikondi kudzera pa Fesibuku | Female | |
CheMbwana wamangidwa pa 12 February 2024 pa kafukufuku amene apolisi ya Mangochi anakhazikitsa | CheMbwana wamangidwa pa twelofu febuluwale twente twente folo pa kafukufuku amene apolisi ya Mangochi anakhazikitsa | Female | |
Polankhula ndi Angaliba mneneri wa polisiyu anati nyamatayu amene amagwiritsa ntchito dzina lakuti Richard Chesani pa Facebook wakhala akuchita ma ubwezi ndi amayi ochuluka | Polankhula ndi Angaliba mneneri wa polisiyu anati nyamatayu amene amagwiritsa ntchito dzina lakuti Ritchadi Chesani pa Fesibuku wakhala akuchita ma ubwezi ndi amayi ochuluka | Female | |
apolisi akhala akulandira madando kuchokera kwa amayi osiyanasiyana mmaboma a Zomba,Mchinji,Machinga ,Lilongwe komanso ena a m'boma lomweli la Mangochi | apolisi akhala akulandira madando kuchokera kwa amayi osiyanasiyana mmaboma a Zomba,Mchinji,Machinga ,Lilongwe komanso ena a m'boma lomweli la Mangochi | Female | |
Chikondi chikafika pa mpondachimera iye amamuuza mkaziyo kuti akumane ku Mangochi, ndipo pompopompo amamutengera ku malo okonza tsitsi | Chikondi chikafika pa mpondachimera iye amamuuza mkaziyo kuti akumane ku Mangochi, ndipo pompopompo amamutengera ku malo okonza tsitsi | Female | |
Akatelo amabwereka phone ya mkaziyo ponama kuti yake yazima ndi ndalama koma omweo samaonekanso.Anatero Daudi | Akatelo amabwereka foni ya mkaziyo ponama kuti yake yazima ndi ndalama koma omweo samaonekanso.Anatero Daudi | Female | |
Mzimayi wina pa 10 February adaberedwa mwa njirayinso ochokera ku Nsanje amene anamubera phone ya mtundu wa Redmi Note 10 ya ndalama zokwana K250,000 | Mzimayi wina pa teni febuluwale adaberedwa mwa njirayinso ochokera ku Nsanje amene anamubera phone ya mtundu wa Redimai Noti teni ya ndalama zokwana thu handiledi andi fifite sauzande kwacha | Female | |
Padakali pano apolisi akwanitsa kupeza wina wa katundu amene M'bwana wakhala akuba. Junior M'bwana amene akufunikanso ndi polisi ya Lilongwe akuyembekezera kukalowa m'bwalo la milandu posachedwapa | Padakali pano apolisi akwanitsa kupeza wina wa katundu amene M'bwana wakhala akuba. Juniyo M'bwana amene akufunikanso ndi polisi ya Lilongwe akuyembekezera kukalowa m'bwalo la milandu posachedwapa | Female | |
Iye amachokera mmudzi mwa Wadali mfumu yaikulu Katuli m'boma la Mangochi. Ku Mangochi apolisi amanga mzibambo wina emwe dzina lake ndi Bamusi Neva wazaka 30 zakubadwa | Iye amachokera mmudzi mwa Wadali mfumu yaikulu Katuli m'boma la Mangochi. Ku Mangochi apolisi amanga mzibambo wina emwe dzina lake ndi Bamusi Neva wazaka fete zakubadwa | Female | |
ndi anthu ena seven pa mlandu oganiziridwa kuti aononga katundu pa malo ochitila chipikisheni pa koche ku Madelco m'bomalo | ndi anthu ena seveni pa mlandu oganiziridwa kuti aononga katundu pa malo ochitila chipikisheni pa koche ku Madeko m'bomalo | Female | |
Mneneri wa apolice ya Mangochi Inspector Amina Tepani Daudi watsimikiza za izi ndipo wati katundu amene wasakazidwa ndiwandalama pafupifupi K745,000 | Mneneri wa apolice ya Mangochi Insipekita Amina Tepani Daudi watsimikiza za izi ndipo wati katundu amene wasakazidwa ndiwandalama pafupifupi seveni handiledi andi fifite sauzande kwacha | Female | |
Malingana ndi inspector Daudi oyendetsa galimoto wina amene dzina Lake ndi Madalitso George anachita ngozi pogunda wanjinga | Malingana ndi inspekita Daudi oyendetsa galimoto wina amene dzina Lake ndi Madalitso Joji anachita ngozi pogunda wanjinga | Female | |
kamba kothamanga kwambiri ndipo wanjingayo wavulala komabe mosadetsa nkhawa. Oyendetsa galimotoyo anathamangira pa malo achipikisheniwo pomwe panali apolisi kukanena za ngoziyo | kamba kothamanga kwambiri ndipo wanjingayo wavulala komabe mosadetsa nkhawa. Oyendetsa galimotoyo anathamangira pa malo achipikisheniwo pomwe panali apolisi kukanena za ngoziyo | Female | |
Koma anthu okwiya anamutsatira kwinaku akumugenda, kwinaku akugenda galimotoyo.Poona mmene zinthu zinalili anathawa ndi galimotoyo kupita ku polisi ya Mangochi | Koma anthu okwiya anamutsatira kwinaku akumugenda, kwinaku akugenda galimotoyo.Poona mmene zinthu zinalili anathawa ndi galimotoyo kupita ku polisi ya Mangochi | Female | |
Apa anthu okwiyawa anayamba kusakaza katundu wapamalopo poganiza kuti amuthawitsa munthuyo mwadala. Kutsatira kafukufuku wa apolisi amanga anthu eight | Apa anthu okwiyawa anayamba kusakaza katundu wapamalopo poganiza kuti amuthawitsa munthuyo mwadala. Kutsatira kafukufuku wa apolisi amanga anthu eiti | Female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.