audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
ndipo akuyembekezera kukayankha mlandu asakaza katundu zomwe ndizosemphana ndi gao 344 la Malamulo
ndipo akuyembekezera kukayankha mlandu asakaza katundu zomwe ndizosemphana ndi gao fili fotefo la Malamulo
Female
Padakali pano inspector Daudi walangiza anthu kuti apewa kutengera malamulo mmanja mwao. M’boma la Nkhotakota akufunafuna a Rhoda Chinganda amene akuwaganizira kuti abaya ndi kupha a Faith Mustafa
Padakali pano insipekita Daudi walangiza anthu kuti apewa kutengera malamulo mmanja mwao. M’boma la Nkhotakota akufunafuna a Roda Chinganda amene akuwaganizira kuti abaya ndi kupha a Fefi Musitafa
Female
powaganizira kuti amachita ubwenzi wa mseri ndi amuna awo. Malingana ndi mneneri wa polisi ya Nkhunga a Andrew Kamanga
powaganizira kuti amachita ubwenzi wa mseri ndi amuna awo. Malingana ndi mneneri wa polisi ya Nkhunga a Andulu Kamanga
Female
Lamulungu lapitali, woganiziridwayu ndi mwamuna wake adapita ku ntchito kwa malemuwa kuti akawafunse za mphekesera zoti akuyenda ndi amuna awo
Lamulungu lapitali, woganiziridwayu ndi mwamuna wake adapita ku ntchito kwa malemuwa kuti akawafunse za mphekesera zoti akuyenda ndi amuna awo
Female
Iwo adati, pomwe amawafunsa za nkhaniyi, mkangano unabuka pakati pa akaziwa ndipo woganiziridwayu adatulutsa chida chakuthwa ndikubaya nacho mzawoyo pachidale kenako n'kuthawa
iwo adati, pomwe amawafunsa za nkhaniyi, mkangano unabuka pakati pa akaziwa ndipo woganiziridwayu adatulutsa chida chakuthwa ndikubaya nacho mzawoyo pachidale kenako n'kuthawa
Female
Kutsatira izi mwamunayo adathamanga pa mudzi wina kukadziwisa anthu za nkhaniyi omwe adathamangira ku malowo ndipo adapeza mayiyu ali magazi okhaokha
Kutsatira izi mwamunayo adathamanga pa mudzi wina kukadziwisa anthu za nkhaniyi omwe adathamangira ku malowo ndipo adapeza mayiyu ali magazi okhaokha
Female
Zotsatira zakuchipatala zawonesa kuti mayiyu wafa kamba kotaya magazi kwambiri. Mu program yathu ya Mindset Change lero half past 9 pa Angaliba Television
Zotsatira zakuchipatala zawonesa kuti mayiyu wafa kamba kotaya magazi kwambiri. Mu pulogalamu yathu ya Maindi seti chenji lero hafu pasiti naini pa Angaliba Televizyoni
Female
tikhale tikukambirana nkhani yokwatilana amuna kapena akazi okhaokha ndi Apostle Innocent Nyirenda a mpingo wa Kingdom Ambassadors International Church. Kuti timve mbali ya zipembezo pa nkhaniyi
tikhale tikukambirana nkhani yokwatilana amuna kapena akazi okhaokha ndi Aposito Inosenti Nyirenda a mpingo wa King’idomu ambasadazi intaneshono tchetchi. Kuti timve mbali ya zipembezo pa nkhaniyi
Female
Kumbukirani Kuti program yi ikhalanso live patsamba lathu la Facebook nthawi yomweyo. Ngati njila imodzi yolimbikisila chipembezo Chachisilamu mdziko muno
Kumbukirani Kuti pulogalamu yi ikhalanso laivi patsamba lathu la fesibuku nthawi yomweyo. Ngati njila imodzi yolimbikisila chipembezo Chachisilamu mdziko muno
Female
anthu ammudzi wa kasambwe group village kadewele mfumu yaikulu mwambo m'boma la Zomba loweluka la pa 23 December 2023
anthu ammudzi wa kasambwe gulupi vileji kadewele mfumu yaikulu mwambo m'boma la Zomba loweluka la pa twente fili disemba twente twente fili
Female
anakonza dawa kapena kuti msonkhano omwe unali pa mutu oti chisilamu chimalimbikisa mtendere
anakonza dawa kapena kuti msonkhano omwe unali pa mutu oti chisilamu chimalimbikisa mtendere
Female
Mwambowu omwe unalemekezedwa ndi anthu monga chairman wakuti southern region kubunge la Qadria Muslim Association of Malawi
Mwambowu omwe unalemekezedwa ndi anthu monga chairman wakuti southern region kubunge la kwadiliya muzilimu asosiyeshoni ofu Malawi
Female
shelkh arhaj Musa juma achair akuchigawo chaku mmawa shelkh arhaj barasani, msungi chuma wa mchigawo chakummawa
shekhi alaji Musa juma tcheya akuchigawo chaku mmawa shekhi alaji barasani, msungi chuma wa mchigawo chakummawa
Female
mafumu , komanso mlendo olemekezeka a National chairman a Qadria Muslim Association of Malawi shelkh Amir Jafali Kawinga, Osaiwalaso nyumba zoulusa mawu monga Radio Islam
mafumu , komanso mlendo olemekezeka a neshono tcheyamani a kwadiliya muzilimu asosiyeshoni ofu Malawi shekhi amilu Jafali Kawinga, Osaiwalaso nyumba zoulusa mawu monga Rediyi isilamu
Female
Angaliba TV komanso radio. Mwazina mkumano unapeleka mpata Kwa anthu apanzikiti wapa kasambwe
Angaliba Tivi komanso rediyo. Mwazina mkumano unapeleka mpata Kwa anthu apanzikiti wapa kasambwe
Female
Omwe anapezelapo mwayi ofotokoza mavuto omwe Iwo ngati asilamu aqadria akukumana nawo pamoyo wawo wa tsiku ndi tsiku
Omwe anapezelapo mwayi ofotokoza mavuto omwe Iwo ngati asilamu akwadiliya akukumana nawo pamoyo wawo wa tsiku ndi tsiku.
Female
Pakuyankhula pawo anakamba zinthu zingapo koma chomwe chinakula nsinkhu inali nkhani ya njala yomwe anapempha a National chairman kuti akapita Kwa akuluakulu ena akathe kukamba za vuto lomwe lawagwela kumalowo
Pakuyankhula pawo anakamba zinthu zingapo koma chomwe chinakula nsinkhu inali nkhani ya njala yomwe anapempha a Neshono tcheyamani kuti akapita Kwa akuluakulu ena akathe kukamba za vuto lomwe lawagwela kumalowo
Female
kupatula za vuto lachakudya anakambanso mavuto ngati kusowa Kwa madzi aukhondo zosiyanasiyana ngati kusowa kwa madzi aukhondo zomwe zikupeleka chiopsezo Kwa anthu a m'delari
kupatula za vuto lachakudya anakambanso mavuto ngati kusowa Kwa madzi aukhondo zosiyanasiyana ngati kusowa kwa madzi aukhondo zomwe zikupeleka chiopsezo Kwa anthu a m'delari
Female
kuti akhonza kudwala nthenda zosiyanasiyana kuphatikizapo Cholera yomwe yavuta mziko muno. Poyankhulapo mfumu kasambwe kuimilira delari Iwo anati asilamu abwelesa ntendele
kuti akhonza kudwala nthenda zosiyanasiyana kuphatikizapo kolela yomwe yavuta mziko muno. Poyankhulapo mfumu kasambwe kuimilira delari Iwo anati asilamu abwelesa ntendele
Female
komanso chitukuko mdela lawo zomwe anaonjezela kuti akapita akuluakulu wa kuntunda ndi ma office ena kukambilana za mavuto omwe anthu akukumana awo
komanso chitukuko mdela lawo zomwe anaonjezela kuti akapita akuluakulu wa kuntunda ndi ma ofesi ena kukambilana za mavuto omwe anthu akukumana awo
Female
monganso nkhani yothandiza azimayi pa machine kuti zitha kusoka komanso azipansidwa mpata womabweleka ngongole zithandiza kutukula delali mmagawo ambiri
monganso nkhani yothandiza azimayi pa matchini kuti zitha kusoka komanso azipansidwa mpata womabweleka ngongole zithandiza kutukula delali mmagawo ambiri
Female
Poyankhulapo mlendo olemekezeka komanso mkulu wa Qadria Muslim Association of Malawi shelkh Amir Jafali Kawinga anati zonse zimene akamba anthu anva
Poyankhulapo mlendo olemekezeka komanso mkulu wa kwadiliya muzilimu asosiyeshoni ofu Malawi shekhi amilu Jafali Kawinga anati zonse zimene akamba anthu anva
Female
ndipo Iwo sangakwanise paokha koma akuyenela kugwilana manja ndi anthu komanso akuluakulu akudelari komaso ndi thandizo la Mulungu zonse ndizotheka
ndipo Iwo sangakwanise paokha koma akuyenela kugwilana manja ndi anthu komanso akuluakulu akudelari komaso ndi thandizo la Mulungu zonse ndizotheka
Female
Aphunzitsi a ma timu a FCB Nyasa Big Bullets ndi Mighty Mukuru Wanderers ati akudziwa zakufunika kwa masewero omwe ali nawo mawa mu ndime ya semifayinolo ya chikho cha Castel
Aphunzitsi a ma timu a efusibi Nyasa Bigi Buletsi ndi Maite Mukuru Wandilazi ati akudziwa zakufunika kwa masewero omwe ali nawo mawa mu ndime ya semifayinolo ya chikho cha Kasotelo
Female
Timu ya Wanderers ikumana ndi timu ya Bullets pamasewero ofuna kuzipezera malo mu ndime yomaliza ya chikhochi
Timu ya Wandilazi ikumana ndi timu ya Buletsi pamasewero ofuna kuzipezera malo mu ndime yomaliza ya chikhochi
Female
Poyankhula ndi Angaliba, m’phunzitsi wamkulu wa timu ya FCB Nyasa Big Bullets, Kalisto Pasuwa wati ngakhale atenga kale zikho ziwiri
Poyankhula ndi Angaliba, m’phunzitsi wamkulu wa timu ya Efusibi Nyasa Bigi Buletsi, Kalisto Pasuwa wati ngakhale atenga kale zikho ziwiri
Female
komabe aliyense ku timuyi akudziwa zakufunikila kopambana ndi Wanderers. Pasuwa anaonjezela kuti akudziwa kuti Wanderers ibwera ndi mtima ofuna kupambana
komabe aliyense ku timuyi akudziwa zakufunikila kopambana ndi Wandilazi. Pasuwa anaonjezela kuti akudziwa kuti Wandilazi ibwera ndi mtima ofuna kupambana
Female
kutengera kuti chaka chino sanapambane chikho chilichonse koma anyamata awo awakonzekelanso kuti azachite bwino. Kumbali yake mphunzitsi wa timu ya Wanderers, Mark Harrison
kutengera kuti chaka chino sanapambane chikho chilichonse koma anyamata awo awakonzekelanso kuti azachite bwino. Kumbali yake mphunzitsi wa timu ya Wandilazi, Maki Halisoni
Female
wati osewera ake akuyenera kuchita chilichonse chotheka kuti apambane masewero'wa. Harrison anatinso pokhapo pokhala kuti chaka chino sanapambane chikho chili chonse
wati osewera ake akuyenera kuchita chilichonse chotheka kuti apambane masewero'wa. Halisoni anatinso pokhapo pokhala kuti chaka chino sanapambane chikho chili chonse
Female
akuyenera kukhala mangolomela kwa osewera ake. Timu yomwe izapambane izakumana ndi timu ya Silver Strikers yomwe lero yagonjetsa timu ya Bangwe All Stars
akuyenera kukhala mangolomela kwa osewera ake. Timu yomwe izapambane izakumana ndi timu ya siliva sitilaikazi yomwe lero yagonjetsa timu ya Bangwe ositazi
Female
ndi zigoli ziwiri kwa duu zomwe anagoletsa ndi Chimwemwe Idana komanso Patrick Macheso. Bungwe la Evidence Action lalimbikitsa anthu kumwa madzi aukhondo
ndi zigoli ziwiri kwa duu zomwe anagoletsa ndi Chimwemwe Idana komanso Patiliki Macheso. Bungwe la evidensi akishoni lalimbikitsa anthu kumwa madzi aukhondo
Female
maka mnyengo ya mvulayi yomwe matenda otsekula mmimba amachuluka. Izi zalankhulidwa ndi Moses Chisangwala emwe ndioyang'anira ntchito za bungweri
maka mnyengo ya mvulayi yomwe matenda otsekula mmimba amachuluka. Izi zalankhulidwa ndi Mozesi Chisangwala emwe ndioyang'anira ntchito za bungweri
Female
polankhula ndi Angaliba pomwe amayankhapo mmene Action Evidence ikuchitila popititsa patsogolo Umoyo wabwino mdziko muno
polankhula ndi Angaliba pomwe amayankhapo mmene akishoni evidensi ikuchitila popititsa patsogolo Umoyo wabwino mdziko muno
Female
Chisangwala anati kugwiritsa ntchito madzi otetezeka ndi njira yokhayo yaikulu yopanga anthu kukhala athanzi labwino pothana ndi matenda otsekula mmimba kuphatikiza Cholera
Chisangwala anati kugwiritsa ntchito madzi otetezeka ndi njira yokhayo yaikulu yopanga anthu kukhala athanzi labwino pothana ndi matenda otsekula mmimba kuphatikiza kolela
Female
Malingana ndi a Chisangwana bungwe lao la Evidence Action Likuika zipangizo zomwe amagwiritsa ntchito kupereka mankhwala a Chlorine mmijigo
Malingana ndi a Chisangwana bungwe lao la Evidence Action Likuika zipangizo zomwe amagwiritsa ntchito kupereka mankhwala a Chlorine mmijigo
Female
Chomcho iwo amema anthu omwe amatunga madzi Mmijigo kuti agwiritse ntchito bwino ndondomekoyi pofuna kukhala ndi moyo wathanzi
Chomcho iwo amema anthu omwe amatunga madzi Mmijigo kuti agwiritse ntchito bwino ndondomekoyi pofuna kukhala ndi moyo wathanzi
Female
Pomaliza a Chisangwala anapempha anthu okhala Mmadera amene ntchitoyi ikugwirika kuti asamalire zipangizo zoperekera mankhwalawo
Pomaliza a Chisangwala anapempha anthu okhala Mmadera amene ntchitoyi ikugwirika kuti asamalire zipangizo zoperekera mankhwalawo
Female
Mmau ake mmodzi mwa anthu amene akupindula ndi ntchitoyi a Mustepher Juma ammudzi mwa Kumbana Mfumu yaikulu Sitola m'boma la Machinga
Mmau ake mmodzi mwa anthu amene akupindula ndi ntchitoyi a Musitafa Juma ammudzi mwa Kumbana Mfumu yaikulu Sitola m'boma la Machinga
Female
anayamikira Bungwe la Evidence Action powabweretsera ndondomekoyi yomwe anati yatukula moyo wao pakuti vuto lamatenda otsekula lachepa
anayamikira Bungwe la evidensi akishoni powabweretsera ndondomekoyi yomwe anati yatukula moyo wao pakuti vuto lamatenda otsekula lachepa
Female
Juma emwe ndi mmodzi mwa oyang'anira mijigo ya mmudzimo anati iwo ndi anthu onse akusamalila zipangozozi kuti zipitilile kuwathandiza
Juma emwe ndi mmodzi mwa oyang'anira mijigo ya mmudzimo anati iwo ndi anthu onse akusamalila zipangozozi kuti zipitilile kuwathandiza
Female
Evidence Action ikugwira ntchito yopereka mankhwala opha tizilombo mmadzi mmaboma a Mangochi,Machinga,Balaka,Zomba,Neno,Chiladzulu,Mwanza ndi Blantyre
Evidensi akishoni ikugwira ntchito yopereka mankhwala opha tizilombo mmadzi mmaboma a Mangochi,Machinga,Balaka,Zomba,Neno,Chiladzulu,Mwanza ndi Bulantaya
Female
Bwalo la milandu lalikulu laonjezera nthawi yomwe chipani cha DPP chingathe kuchititsa convention. Mwezi wa September oweluza Simeon Mdeza
Bwalo la milandu lalikulu laonjezera nthawi yomwe chipani cha Dipipi chingathe kuchititsa conveshoni. Mwezi wa Sepitemba oweluza Simiyoni Mdeza
Female
adagamula kuti chipanichi chichititse msonkhano waukuluwu pasanathe masiku 90 kuyambira patsikulo pomwe padali pa 28 September 2023
adagamula kuti chipanichi chichititse msonkhano waukuluwu pasanathe masiku nainte kuyambira patsikulo pomwe padali pa twente eiti sepitemba twente twente fili
Female
Izi zinakakamiza chipanichi kukonza masiku a pa 26 ndi 27 December 2023 mofuna kugwirizana ndi chigamulocho
Izi zinakakamiza chipanichi kukonza masiku a pa twente sikisi ndi twente seveni Disemba twente twente fili mofuna kugwirizana ndi chigamulocho
Female
Kutsatira chigamulo chatsopanocho DPP kudzera mu Mkalata yomwe yosainidwa ndi olankhulira Shadrick Namalomba ati panopa aimitsa kaye dongosolo la pa 26 ndi 27 kufikira mtsogolo
Kutsatira chigamulo chatsopanocho Dipipi kudzera mu Mkalata yomwe yosainidwa ndi olankhulira Shadileki Namalomba ati panopa aimitsa kaye dongosolo la pa twente sikisi ndi twente seveni kufikira mtsogolo
Female
pomwe adzalengezenso akasumbana mitu. Padakali pano anthu omwe adabwera poyera kufuna kudzapikisana pa mpando otsogolela chipanichi ndi a Kondwani Nankhumwa ndi a Peter Munthalika
pomwe adzalengezenso akasumbana mitu. Padakali pano anthu omwe adabwera poyera kufuna kudzapikisana pa mpando otsogolela chipanichi ndi a Kondwani Nankhumwa ndi a Pita Munthalika
Female
Mwezi wa September oweluza Simeon Mdeza adagamula kuti chipanichi chichititse msonkhano waukuluwu pasanathe masiku 90 kuyambira patsikulo pomwe padali pa 28 September 2023
Mwezi wa Sepitemba oweluza Simiyoni Mdeza adagamula kuti chipanichi chichititse msonkhano waukuluwu pasanathe masiku nainte kuyambira patsikulo pomwe padali pa twente eiti Sepitemba twente twente fili
Female
M’modzi mwa akatswiri oimba a mdziko muno Jafali Thom yemwe amkaimba mu gulu la Fikisa wamwalira
M’modzi mwa akatswiri oimba a mdziko muno Jafali Thomu yemwe amkaimba mu gulu la Fikisa wamwalira
Female
Oimbayu yemwe adadziwika bwino ndi nyimbo monga Ademwiche, Nantchengwa, Akamwire ndi zina zambiri. Watsimikiza za imfayi mmodzi wa oimba yemwe amakhala ndi malemuyu kwa Ntopwa ku Bangwe
Oimbayu yemwe adadziwika bwino ndi nyimbo monga Ademwiche, Nantchengwa, Akamwire ndi zina zambiri. Watsimikiza za imfayi mmodzi wa oimba yemwe amakhala ndi malemuyu kwa Ntopwa ku Bangwe
Female
mu mzinda wa Blantyre ndipo wati Thom wamwalira m’bandakucha wa lero atadwala nthawi yochepa ku Ntaja m’boma la Machinga
mu mzinda wa Bulantaya ndipo wati Thomu wamwalira m’bandakucha wa lero atadwala nthawi yochepa ku Ntaja m’boma la Machinga
Female
Gulu la anthu lomwe limazitcha kuti Friends of Atupele Muluzi lapempha anthu dziko muno kuti asiye kuchita zionesero koma kuti apeze munthu yemwe angazathe kupulumusa dziko lino yemwe ati ndi Atupele Muluzi yekha
Gulu la anthu lomwe limazitcha kuti Fulenzi ofu Atupele Muluzi lapempha anthu dziko muno kuti asiye kuchita zionesero koma kuti apeze munthu yemwe angazathe kupulumusa dziko lino yemwe ati ndi Atupele Muluzi yekha
Female
Izi zayankhulidwa ndi mlembi wa mkulu wa gululi yemwe ndi Stain Chidothi ku mkumano wa atolankhani omwe anakonza ku Blantyre Lodge pa 14 December 2023
Izi zayankhulidwa ndi mlembi wa mkulu wa gululi yemwe ndi Siteni Chidothi ku mkumano wa atolankhani omwe anakonza ku Bulantaya loji pa fotini Disemba twente twente fili
Female
Chidothi wati Atupele Muluzi yekha ndi yemwe Ali ndi kuthekela kozapulumusa dziko lino ku mavuto omwe likukumanawo nawo monga kuchepesedwa mphamvu Kwa ndalama ya kwacha mwa Zina
Chidothi wati Atupele Muluzi yekha ndi yemwe Ali ndi kuthekela kozapulumusa dziko lino ku mavuto omwe likukumanawo nawo monga kuchepesedwa mphamvu Kwa ndalama ya kwacha mwa Zina
Female
Anapilizanso kupempha anthu dziko muno kuti azavotele munthu yemwe ali ndi kuthekela komanso yemwe alibe mantha Gulu la friends of Atupele Muluzi tsopano lakwanisa chaka chimodzi chikhazikisidwileni
Anapilizanso kupempha anthu dziko muno kuti azavotele munthu yemwe ali ndi kuthekela komanso yemwe alibe mantha Gulu la fulenzi ofu Atupele Muluzi tsopano lakwanisa chaka chimodzi chikhazikisidwileni
Female
Bungwe la Football Association of Malawi lati zonse zokonzekera chisankho chomwe chichitike pa 16, pa 16 December 2023 ku Mzuzu hotel zili m'chimake
Bungwe la futubo asosiyeshoni ofu Malawi lati zonse zokonzekera chisankho chomwe chichitike pa sikisitini, pa sikisitini Disemba twente twente fili ku Mzuzu hotelo zili m'chimake
Female
M'modzi mwa akulu akulu omwe ayendetse chisankhochi a James Masumbu ati zikalata zovotera zakonzedwa kale komaso onse omwe adzaponye nawo voti adzapatsidwa zowayenereza
M'modzi mwa akulu akulu omwe ayendetse chisankhochi a Jemusi Masumbu ati zikalata zovotera zakonzedwa kale komaso onse omwe adzaponye nawo voti adzapatsidwa zowayenereza
Female
kuti adzazindikilidwe patsiku lovotali. Iwo apitiliza kunena kuti chitetezo chakhwimitsidwa pomwe ayika apolisi ochuluka omwe adzakhale akupereka chitetezo patsikuli
kuti adzazindikilidwe patsiku lovotali. Iwo apitiliza kunena kuti chitetezo chakhwimitsidwa pomwe ayika apolisi ochuluka omwe adzakhale akupereka chitetezo patsikuli
Female
komaso achepetsa nambala ya anthu ongobwera kudzaonera masankhowa ndipo adzalola okhawo omwe akupikisana kuti adzabweretse mlendo m'modzi yekha aliyense
komaso achepetsa nambala ya anthu ongobwera kudzaonera masankhowa ndipo adzalola okhawo omwe akupikisana kuti adzabweretse mlendo m'modzi yekha aliyense
Female
Pa chisankhochi a Walter Nyamilandu manda ndiwomwe adzapikisane ndi Fleetwood Hayiya pa mpando wawu president. Mipando ina yomwe anthu apikisane ndi wachiwiri kwa mtsogoleri komanso mamembala a komiti yayikulu ya bungweri
Pa chisankhochi a Wota Nyamilandu manda ndiwomwe adzapikisane ndi Fulitihudu Hayiya pa mpando wawu pulezidenti. Mipando ina yomwe anthu apikisane ndi wachiwiri kwa mtsogoleri komanso mamembala a komiti yayikulu ya bungweri
Female
Chipani cha DPP chakonza pa 26 December kukhala tsiku lomwe lichititse msonkhano wosankha adindo a chipanichi. Izi zikudza kutsatila mkumano wa National Governing Council wa chipanichi omwe wachitika ku Mangochi
Chipani cha Dipipi chakonza pa twente sikisi Disemba kukhala tsiku lomwe lichititse msonkhano wosankha adindo a chipanichi. Izi zikudza kutsatila mkumano wa Neshono gavaning’I Khanso wa chipanichi omwe wachitika ku Mangochi
Female
Mumkumanowo Munthalika wapempha anthu omwe akufuna kudzapikisana kuti asunge bata.Ndipo a Munthalika ati azapilisana nao
Mumkumanowo Munthalika wapempha anthu omwe akufuna kudzapikisana kuti asunge bata.Ndipo a Munthalika ati azapilisana nao
Female
Mkokemkoke ukupitililabe ku chipani cha DPP pomwe mtsogoleri wa chipanichi pro Peter Munthalika wachotsa a Kondwani Nankhumwa pa udindo wa wachiwiri wa mtsogoleri wa chipanichi mchigao chakummwela
Mkokemkoke ukupitililabe ku chipani cha Dipipi pomwe mtsogoleri wa chipanichi pro Pita Munthalika wachotsa a Kondwani Nankhumwa pa udindo wa wachiwiri wa mtsogoleri wa chipanichi mchigao chakummwela
Female
A Munthalika akhazika a Nankhumwa kukhala mlangizi wao pamodzi ndi a Paul Gadama komanso a Cecilia Chazama. Malingana ndi kalata yomwe Angaliba yaona
A Munthalika akhazika a Nankhumwa kukhala mlangizi wao pamodzi ndi a Po Gadama komanso a Sisiliya Chazama. Malingana ndi kalata yomwe Angaliba yaona
Female
a Munthalika apanga izi kugwiritsa ntchito mphanvu za malamulo chipanichi gao 10 sub section 8 lomwe limapereka mphanvu kwa mtsogoleri wa chipani kusankha adindo
a Munthalika apanga izi kugwiritsa ntchito mphanvu za malamulo chipanichi gao teni sabu sekishoni eiti lomwe limapereka mphanvu kwa mtsogoleri wa chipani kusankha adindo
Female
Kotelo iwo aika a George Chaponda pa mpando wa wachiwiri wa mtsogoleri wa chipanichi mchigao chakummwela ndipo a Mary Navitcha asankhidwa kukhala oyang'anira a mayi mchipani
Kotelo iwo aika a Joji Chaponda pa mpando wa wachiwiri wa mtsogoleri wa chipanichi mchigao chakummwela ndipo a Mele Navitcha asankhidwa kukhala oyang'anira a mayi mchipani
Female
Komatu pangopita nthawi yochepa chabe pomwe a Grelzeder Jeffrey amene anachotsedwanso pa mpando wa Mlembi akagogoda ku bwalo la milandu pofuna kuletsa a Munthalika kuwasintha pa udindowu
Komatu pangopita nthawi yochepa chabe pomwe a Gilezeda jefule amene anachotsedwanso pa mpando wa Mlembi akagogoda ku bwalo la milandu pofuna kuletsa a Munthalika kuwasintha pa udindowu
Female
Pomwe kunsamvana mchipani cha DPP kwayala mphasa,Mlembi wa chipanichi Grezelder Jeffrey wakamang'ala ku bwalo la milandu pakuchotsedwa kakwe pampando
Pomwe kunsamvana mchipani cha Dipipi kwayala mphasa,Mlembi wa chipanichi Gilezeda jefule wakamang'ala ku bwalo la milandu pakuchotsedwa kakwe pampando
Female
Masiku apitawa mtsogoleri wa chipani cha DPP Professor Peter Munthalika anachotsa udindo a Jeffrey ndikuwapatsa udindo wa wachiwiri wa mtsogoleri wa chipanichi mchigao chapakati
Masiku apitawa mtsogoleri wa chipani cha Dipipi Pulofesa Pita Munthalika anachotsa udindo a Jefule ndikuwapatsa udindo wa wachiwiri wa mtsogoleri wa chipanichi mchigao chapakati
Female
ndipo mmalo mwao paudindo wa Mlembi wamkulu adaikapo Dr Clement Mwale. Koma a Jeffrey akudana ndi izi ndipo iwo akufunanso khoti liletse Dr Clement Mwale kugwira ntchito ngati Mlembi wa chipanichi
ndipo mmalo mwao paudindo wa Mlembi wamkulu adaikapo Dokota Kilementi Mwale. Koma a Jefule akudana ndi izi ndipo iwo akufunanso khoti liletse Dokota Kilementi Mwale kugwira ntchito ngati Mlembi wa chipanichi
Female
Pakadali pano bwalo lalikulu la milandu mu mzinda wa Lilongwe laika lachiwiri likubwerali kukhala tsiku lakumva Mulanduwu kuyambira nthawi ya 2 koloko masana
Pakadali pano bwalo lalikulu la milandu mu mzinda wa Lilongwe laika lachiwiri likubwerali kukhala tsiku lakumva Mulanduwu kuyambira nthawi ya thu koloko masana
Female
DPP yati ichititsa mkumano wa Nation Governing Council Lachitatu sabata yamawa pa 13 December 2023
Dipipi yati ichititsa mkumano wa Neshoni gavaning’I khanso Lachitatu sabata yamawa pa fetini Disemba twente twente fili
Female
Izi ndimalinga ndi kalata yomwe chipanichi chatulutsa chosayinidwa ndi Mlembi wa Administration ya DPP, Francis Mphepo
Izi ndimalinga ndi kalata yomwe chipanichi chatulutsa chosayinidwa ndi Mlembi wa adiminisitileshoni ya Dipipi, Fulansisi Mphepo
Female
Mkumanowu udzakachitikira ku Nkopola lodge m'boma la Mangochi. Kalatayi yatulutsidwa kutsatira mkumano waukulu wa Central Executive committee
Mkumanowu udzakachitikira ku Nkopola loji m'boma la Mangochi. Kalatayi yatulutsidwa kutsatira mkumano waukulu wa sentilo ekizekitivi komiti
Female
omwe unachitika Loweluka pa 9 December 2023 ku Mangochi komwe atolankhani sanaloledwe kulowa
omwe unachitika Loweluka pa naini Disemba twente twente fili ku Mangochi komwe atolankhani sanaloledwe kulowa
Female
Koma Angaliba yapeza kuti anthu ena amene anaenera kukhala ku zokambiranazo za Central Executive committee sanapezekeko
Koma Angaliba yapeza kuti anthu ena amene anaenera kukhala ku zokambiranazo za sentilo ekizekitivi komiti sanapezekeko
Female
Anamizila kukomoka Kapena Akomokadi Zikuchutika ku NRB Blantyre panopa. Mayi amene mukumuona wagona apayu anaba phone ya mzimayi mzake nkuibisa mu pant
Anamizila kukomoka Kapena Akomokadi Zikuchutika ku enialabi Bulantaya panopa. Mayi amene mukumuona wagona apayu anaba foni ya mzimayi mzake nkuibisa mu panti
Female
Obeledwayo ataona phone yake yasowa, azimayi anagwirizana zoti asechane onse. Ananyamulana kupita ku toilet kukafufuzana. Mpamene adayipeza phone yo mu panti wa mayiwa
Obeledwayo ataona foni yake yasowa, azimayi anagwirizana zoti asechane onse. Ananyamulana kupita ku toileti kukafufuzana. Mpamene adayipeza foni yo mu panti wa mayiwa
Female
Atangoyipeza iwowa adzigwetsa pansi pakadali pano alichikomokere kuseri kwa toilet konko. Ena ati mayiwo sadakomoke koma mwina ndi manyazi
Atangoyipeza iwowa adzigwetsa pansi pakadali pano alichikomokere kuseri kwa toileti konko. Ena ati mayiwo sadakomoke koma mwina ndi manyazi
Female
Komanso ena ati atha kukhala akomokadi. Palibe waamenya ayi. Agwa okha. Ndipo popeza atha kukhala akomokadi, anthu akuopa kuwamenya mwina atha kupitilila nde nzovuta
Komanso ena ati atha kukhala akomokadi. Palibe waamenya ayi. Agwa okha. Ndipo popeza atha kukhala akomokadi, anthu akuopa kuwamenya mwina atha kupitilila nde nzovuta
Female
Kumanyadirako luso lomwe tili nalo. Amene wavulila izi panja pa Bank yi akatenge chifukwa ena atha kutolapo. Mapemphelo ako ayamba kugwila ntchito Mapemphero ako akayamba kugwira ntchito
Kumanyadirako luso lomwe tili nalo. Amene wavulila izi panja pa Banki yi akatenge chifukwa ena atha kutolapo. Mapemphelo ako ayamba kugwila ntchito Mapemphero ako akayamba kugwira ntchito
Female
umangoona anthu ena ayamba kukwiya nawe usanawalakwire chiichonse. Limbikiran kupemphera kuti yemwe sakondera nd moyo wanu, sakondwera nd success yanu akwiye zenizeni chaka chino
umangoona anthu ena ayamba kukwiya nawe usanawalakwire chiichonse. Limbikiran kupemphera kuti yemwe sakondera nd moyo wanu, sakondwera nd sakisesi yanu akwiye zenizeni chaka chino
Female
Ukasamuka mnyumba mwa makolo nkuyamba kukhala wekha mpamene umadziwa kufunika kwawo amayi ako. Mpamene umayamba kumvetsetsa zonse zimene akuchitila pa moyo wako
Ukasamuka mnyumba mwa makolo nkuyamba kukhala wekha mpamene umadziwa kufunika kwawo amayi ako. Mpamene umayamba kumvetsetsa zonse zimene akuchitila pa moyo wako
Female
Achina Gattah Ase walila mu nyimbo ya 'AMA' atakumana ndizikhomo moyo wokhala ekha. Pali ena akukagula machesi ati akufuna awaotche chala awone
Achina Gata Ase walila mu nyimbo ya 'AMA' atakumana ndizikhomo moyo wokhala ekha. Pali ena akukagula machesi ati akufuna awaotche chala awone
Female
Pali ena akukagula machesi ati akufuna awaotche chala awone, Akadzuka mpamene atayambe kuwamenya. Mumva m'mene zithele
Pali ena akukagula machesi ati akufuna awaotche chala awone, Akadzuka mpamene atayambe kuwamenya. Mumva m'mene zithele
Female
angoyesa kuwabwenzela phone anabayo kuti ikhale yao aone ngati sadzuka nkulandira. Ayambe kuwagiligisha. Koma kumalawi kuli luso
angoyesa kuwabwenzela foni anabayo kuti ikhale yao aone ngati sadzuka nkulandira. Ayambe kuwagiligisha. Koma kumalawi kuli luso
Female
Muyese kuwatokosa kukhutu ndika udzu kena kake, simene atalumphiremo. Zimatheka kufusira pano Nde ukatero ujambulenso malo omwe anali phonewo tikumanapo uwona Akufanana ndi winawake
Muyese kuwatokosa kukhutu ndika udzu kena kake, simene atalumphiremo. Zimatheka kufusira pano Nde ukatero ujambulenso malo omwe anali foniwo tikumanapo uwona Akufanana ndi winawake
Female
Koma ine ndingamudzidzimutse nalo khofitu. Akufanana ndi winawake Koma ine ndingamudzidzimutse nalo khofitu ngatinso angachedwe kuuka nkumene. Avuleni nsalu adzidzimuka
Koma ine ndingamudzidzimutse nalo khofitu. Akufanana ndi winawake Koma ine ndingamudzidzimutse nalo khofitu ngatinso angachedwe kuuka nkumene. Avuleni nsalu adzidzimuka
Female
Nde osationesa komwe anabisako bwanji. Atangoti avulidwe zovala apitidwe mphepo Ngati munayesa kwagiligisha osadzuka tayesani kuwakanda kuphaziko. ija imafunika ukhale ochenjera
Nde osationesa komwe anabisako bwanji. Atangoti avulidwe zovala apitidwe mphepo Ngati munayesa kwagiligisha osadzuka tayesani kuwakanda kuphaziko. ija imafunika ukhale ochenjera
Female
Koma nde taonani apapa zomwe zachitikazi olo akapita kunyumba amuna awo azikauza kuti chani ndi ana omwe. Amayi adanamizila kukomoka aja adzuka tsopano
Koma nde taonani apapa zomwe zachitikazi olo akapita kunyumba amuna awo azikauza kuti chani ndi ana omwe. Amayi adanamizila kukomoka aja adzuka tsopano
Female
Anthu ena amtima wabwino adawawuza alichikomokele kuti akadzuka sawamenya ndipo awakwezetsa njinga adzipita kunyumba
Anthu ena amtima wabwino adawawuza alichikomokele kuti akadzuka sawamenya ndipo awakwezetsa njinga adzipita kunyumba
Female
Mpaka anayitanadi njinga ija ndipo itafika mpamene mayi wo adazizimuka nkuyikwela. Zilikoliko m'ma tchalitchi pamene ena awachotsa chiwanda cha mchiuno
Mpaka anayitanadi njinga ija ndipo itafika mpamene mayi wo adazizimuka nkuyikwela. Zilikoliko m'ma tchalitchi pamene ena awachotsa chiwanda cha mchiuno
Female
Anthu ofuna ziphaso zoyendera passport adandaula ndi momwe office ya Immigration ikugwilira ntchito zake ku Lilongwe
Anthu ofuna ziphaso zoyendera pasipoti adandaula ndi momwe ofesi ya Imigileshoni ikugwilira ntchito zake ku Lilongwe
Female
Ena mwa anthu omwe Angaliba inalankhula nawo , atiuza kuti akhala akuyendera kuti atenge ziphaso zawo Kwa nthawi yaitali koma sanatengebe
Ena mwa anthu omwe Angaliba inalankhula nawo , atiuza kuti akhala akuyendera kuti atenge ziphaso zawo Kwa nthawi yaitali koma sanatengebe
Female
John Mfwethu , anati wakhala akuyendera Kwa masabata awiri tsopano kuti apeze chiphaso chake choyendera Iye anati zikudabwitsa kuti anthu ena akabwera tsiku lomwelo amatenga ziphaso zawo
Joni Mfwethu , anati wakhala akuyendera Kwa masabata awiri tsopano kuti apeze chiphaso chake choyendera Iye anati zikudabwitsa kuti anthu ena akabwera tsiku lomwelo amatenga ziphaso zawo
Female
zomwe zikuonetsa kuti akumalipira ndalama ina pamwamba kuti atenge ziphaso zawo. Chipani cha DPP chati ndi chokhudzidwa ndi imfa ya a mayi awo a Salila mdala
zomwe zikuonetsa kuti akumalipira ndalama ina pamwamba kuti atenge ziphaso zawo. Chipani cha Dipipi chati ndi chokhudzidwa ndi imfa ya a mayi awo a Salila mdala
Female
omwe aikidwa mmanda lachiwiri pa 5 December 2023. Mayiwa anamwalila Lolemba kamba kodwala nthenda yothamanga magazi komanso kufa ziwalo
omwe aikidwa mmanda lachiwiri pa faifi Disemba twente twente fili. Mayiwa anamwalila Lolemba kamba kodwala nthenda yothamanga magazi komanso kufa ziwalo
Female
Mmau ake Bright Nsaka amene analankhula mmalo mwa chipani cha DPP anati DPP imayamikira ntchito zochokera kubanja la Mdala kotelo kuferedwa kwao kwakhudzanso chipanichi
Mmau ake Bulaiti Nsaka amene analankhula mmalo mwa chipani cha Dipipi anati Dipipi imayamikira ntchito zochokera kubanja la Mdala kotelo kuferedwa kwao kwakhudzanso chipanichi
Female
Nsaka anati ngakhale mtsogoleri wao Professor Peter Munthalika anachiona chanzelu kukhala nao pamalilowa. Mtsogoleri wakale wa dzikolinoyu anapepesa ndi ndalama yokwana K600,000
Nsaka anati ngakhale mtsogoleri wao Professor Pita Munthalika anachiona chanzelu kukhala nao pamalilowa. Mtsogoleri wakale wa dzikolinoyu anapepesa ndi ndalama yokwana sikisi handiledi sauzande kwacha
Female
Ena mwa akulu a chipani cha DPP omwe analinao pa mwambo wamalilowo ndi Regional governor wa chigao chakummawa Imran Ntenje,Eluby Kandeu amene amayang'anira a mayi mchipanichi
Ena mwa akulu a chipani cha Dipipi omwe analinao pa mwambo wamalilowo ndi lijono gavana wa chigao chakummawa Imulani Ntenje,Elube Kandeu amene amayang'anira a mayi mchipanichi
Female
phungu wa nyumba yamalamulo wa Mangochi central Victoria Kingston,komanso wofalitsa nkhani za chipani cha DPP Shadrick Namalomba
phungu wa nyumba yamalamulo wa Mangochi sentilo vikitoliya king’isitoni,komanso wofalitsa nkhani za chipani cha Dipipi Shadileki Namalomba
Female