audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Mayiwa omwe anali gulupu Nsukamwere amwalila ali ndi zaka 87 zakubadwa. Mtsogoleri wakale wadziko lino Professor Peter Mutharika
Mayiwa omwe anali gulupu Nsukamwere amwalila ali ndi zaka eite seveni zakubadwa. Mtsogoleri wakale wadziko lino pulofesa pita Mutharika
Female
wafika ku mwambo wa maliro a amayi awo a bambo Salire Mdala omwe ndi mmodzi mwa akulu akulu a chipani cha DPP
wafika ku mwambo wa maliro a amayi awo a bambo Salire Mdala omwe ndi mmodzi mwa akulu akulu a chipani cha Dipipi
Female
Zonse zikuchitikira kunyumba kwa Malemuwa mmudzi mwa mwanyama Mfumu yaikulu Mponda kufupi ndi bwalo lalikulu la masewero la Mangochi
Zonse zikuchitikira kunyumba kwa Malemuwa mmudzi mwa mwanyama Mfumu yaikulu Mponda kufupi ndi bwalo lalikulu la masewero la Mangochi
Female
Ena mwa omwe afikanso ndi wachiwiri wa pampando ku chipani cha DPP kuchigawo cha kummawa a Bright Msaka, wofalitsa nkhani ku chipanichi a Shadreck Namalomba,komanso gavanala wa chipanichi
Ena mwa omwe afikanso ndi wachiwiri wa pampando ku chipani cha Dipipi kuchigawo cha kummawa a Bulaiti Msaka, wofalitsa nkhani ku chipanichi a Shadileki Namalomba,komanso gavanala wa chipanichi
Female
ku chigawo cha kummawa a Sheikh Imran Mtenje kungotchulapo ochepa. Mayiwa adamwalira lolemba atadwala kwa kanthawi matenda wothamanga magazi komanso kufa ziwalo
ku chigawo cha kummawa a Shekhi Iimulani Mtenje kungotchulapo ochepa. Mayiwa adamwalira lolemba atadwala kwa kanthawi matenda wothamanga magazi komanso kufa ziwalo
Female
Zina ukanva kamba anga mwaladi ndithu.Ku Monkey_Bay M'boma la Mangochi bambo wina wanjatidwa ndi apolisi chifukwa chovulaza mayi wina pomuluma milomo
Zina ukanva kamba anga mwaladi ndithu.Ku Monkibe M'boma la Mangochi bambo wina wanjatidwa ndi apolisi chifukwa chovulaza mayi wina pomuluma milomo
Female
Mneneli wa polisi ku Monkey Bay Sergeant Alice Sichali watsimikizira Angaliba zankhaniyo ndipo wati izi zachitika usiku wa pa 3 December 2023
Mneneli wa polisi ku Monkibe sajenti Alisi Sichali watsimikizira Angaliba zankhaniyo ndipo wati izi zachitika usiku wa pa fili Disemba twente twente fili
Female
Bamboyu Gift Mulangiwa wa zaka 19 anapita kukaba mnyumba ya Cecelia Musa wa zaka 28 zakubadwa yemwe amachita rent pa malo ena ogona alendo ku dela la Nsaka
Bamboyu Gifiti Mulangiwa wa zaka naintini anapita kukaba mnyumba ya sisiliya Musa wa zaka twente eiti zakubadwa yemwe amachita lenti pa malo ena ogona alendo ku dela la Nsaka
Female
Sichali anati mayiyu atamva phokoso la chilendo anadzuka ndikugwira mbavayi, apa mkuluyo kamba kakuchepa nthanana anangoganiza zoluma mlomo wa mayiyo kuti athawe
Sichali anati mayiyu atamva phokoso la chilendo anadzuka ndikugwira mbavayi, apa mkuluyo kamba kakuchepa nthanana anangoganiza zoluma mlomo wa mayiyo kuti athawe
Female
Atafuula mzimayiyu anthu anabwera ndikugwira bamboyu kenaka anamutengera ku polisi yaying'ono ya Nsaka
Atafuula mzimayiyu anthu anabwera ndikugwira bamboyu kenaka anamutengera ku polisi yaying'ono ya Nsaka
Female
Malingana ndi Sichali mayiyu akulandira thandizo la mankhwala pa chipatala cha Monkey Bay pomwe bamboyu akuyembekezeka kukayankha mlandu othyola nyumba ndi kuvulaza munthu
Malingana ndi Sichali mayiyu akulandira thandizo la mankhwala pa chipatala cha Monkibe pomwe bamboyu akuyembekezeka kukayankha mlandu othyola nyumba ndi kuvulaza munthu
Female
Gift Mulangiwa amachokera mmudzi wa Saiti mdera la mfumu yayikulu Nankumba mboma la Mangochi
Gifiti Mulangiwa amachokera mmudzi wa Saiti mdera la mfumu yayikulu Nankumba mboma la Mangochi
Female
Pomwe dziko la Malawi likudalila kwambiri atolankhani pamauthenga ofunika, Mkhalakale pa nkhani zamalonda Dr Thomson Mpinganjira
Pomwe dziko la Malawi likudalila kwambiri atolankhani pamauthenga ofunika, Mkhalakale pa nkhani zamalonda Dokota Thomusoni Mpinganjira
Female
wapempha atolankhaniwa kuika chidwi kupeza njira zodzidalila pa chuma mmagulu awo. Iwo anati ngati atolankhani akhale ozidalila angakwanitse kugwira ntchito Yao bwino opanda chowasokoneza
wapempha atolankhaniwa kuika chidwi kupeza njira zodzidalila pa chuma mmagulu awo. Iwo anati ngati atolankhani akhale ozidalila angakwanitse kugwira ntchito Yao bwino opanda chowasokoneza
Female
DR Mpinganjira amalankhula izi pa mkumano wapachaka wa gulu la atolankhani la Southern Region Press Club omwe ukuchitikira ku Blantyre
Dokota Mpinganjira amalankhula izi pa mkumano wapachaka wa gulu la atolankhani la Sauveni lijoni pulesi kalabu omwe ukuchitikira ku Bulantaya
Female
Mwazina iwo alimbikitsa gululi kupeza njira zopezera chuma. Mkumanowu omwe uperekenso mwayi kwa atengambali kusankha adindo a gululi, wayamba lachisanuli
Mwazina iwo alimbikitsa gululi kupeza njira zopezera chuma. Mkumanowu omwe uperekenso mwayi kwa atengambali kusankha adindo a gululi, wayamba lachisanuli
Female
ndipo utha laweluka pa 2 December 2023. Timu ya Silver strikers yagonjetsa timu ya Ekwendeni United ndi zigoli zisanu ndi ziwiri Kwa chimodzi mu chikho cha castle
ndipo utha laweluka pa thu Disemba twente twente fili. Timu ya siliva sitilaikazi yagonjetsa timu ya Ekwendeni yunaitedi ndi zigoli zisanu ndi ziwiri Kwa chimodzi mu chikho cha kasitelo
Female
M'phunzitsi wa Ekwendeni United Luka Kalinga wavomereza kuti anyamata ake sadasewere bwino ngakhale kuti anayamba ndi mphavu
M'phunzitsi wa Ekwendeni yunaitedi Luka Kalinga wavomereza kuti anyamata ake sadasewere bwino ngakhale kuti anayamba ndi mphavu
Female
Wachiwiri Kwa m'phunzitsi wa Silver strikers Peter Mgangira anati , anali masewero abwino sayembekeze kupambana popeza anyamata ake ayamba mwachibwana
Wachiwiri Kwa m'phunzitsi wa siliva sitilaikazi pita Mgangira anati , anali masewero abwino sayembekeze kupambana popeza anyamata ake ayamba mwachibwana
Female
Pomwe timu ya FCB Nyasa Bullets yafika mu ndime yomaliza ya chikho cha TNM itagonjetsa timu ya Karonga pa bwalo la Karonga
Pomwe timu ya efusibi Nyasa Buletsi yafika mu ndime yomaliza ya chikho cha Tieniemu itagonjetsa timu ya Karonga pa bwalo la Karonga
Female
FCB Nyasa Bullets tsopano yumana ndi Silver strikers pa 3 December mu final ya TNM super league pa Kamuzu Stadium
Efusibi Nyasa Buletsi tsopano yumana ndi siliva sitilaikazi pa fili Disemba mu faino ya Tieniemu supa ligi pa Kamuzu Sitediyamu
Female
Zionetselo zomwe zinakonzedwa ndi gulu la Malawi First motsogozedwa ndi Bon Kalindo ku Mangochi zatha. Mmau ake Kalindo wapempha adindo
Zionetselo zomwe zinakonzedwa ndi gulu la Malawi Fesiti motsogozedwa ndi Boni Kalindo ku Mangochi zatha. Mmau ake Kalindo wapempha adindo
Female
kuti ayitanitse zisankho mwachangu zamtsogoleli wadziko ponena kuti Dr Lazarus Chakwera alephera. Kalindo wati amalawi adanamizidwa
kuti ayitanitse zisankho mwachangu zamtsogoleli wadziko ponena kuti Dokota Lazalasi Chakwera alephera. Kalindo wati amalawi adanamizidwa
Female
Mumkuyenda kwao Chipwirikiti chinabuka pomwe mkulu wina osadziwikana bwino anafika ndikumakalipila Otsogolela Zionetselo Bon Kalindo
Mumkuyenda kwao Chipwirikiti chinabuka pomwe mkulu wina osadziwikana bwino anafika ndikumakalipila Otsogolela Zionetselo Boni Kalindo
Female
Apa zinapangisa kuti anyamata azitho omwe amapereka chitetezo amugwiregwire mkuluyo. Kalindo analimbikitsabe anthuwa kuti ayende mwa bata
Apa zinapangisa kuti anyamata azitho omwe amapereka chitetezo amugwiregwire mkuluyo. Kalindo analimbikitsabe anthuwa kuti ayende mwa bata
Female
Komabe pomwe zionetselozi zatha anthu ena akugenda ndipo apolisi aphulitsa utsi okhetsa misozi. Achitetezo aboma anali owelengeka pazionetselozi
Komabe pomwe zionetselozi zatha anthu ena akugenda ndipo apolisi aphulitsa utsi okhetsa misozi. Achitetezo aboma anali owelengeka pazionetselozi
Female
Atapangitsa Zionetselo ku chigao chakummwela, chigao chapakati ndi ku mpoto,kutsatila kugwa mphanvu kwa ndalama ya Kwacha, Bon Kalindo alinso Ku Mangochi Kuchititsanso Zionetselo zina
Atapangitsa Zionetselo ku chigao chakummwela, chigao chapakati ndi ku mpoto,kutsatila kugwa mphanvu kwa ndalama ya Kwacha, Boni Kalindo alinso Ku Mangochi Kuchititsanso Zionetselo zina
Female
Unduna wazaumoyo watsimikiza kuti munthu m'modzi wapazeka ndi nthenda ya Anthrax m'dziko muno. Malingana kalata yomwe yasayinidwa ndi mlembi wamkulu mu undunawu Dr Samson Mndolo
Unduna wazaumoyo watsimikiza kuti munthu m'modzi wapazeka ndi nthenda ya Anfilakisi m'dziko muno. Malingana kalata yomwe yasayinidwa ndi mlembi wamkulu mu undunawu Dokota Samusoni Mndolo
Female
munthuyu wapezeka ndi nthendayi pachipatala china m'boma la Mzimba ndipo zotsatira zake zatsimikizika lolemba sabata ino ndi nthambi ya Public Health Institute of Malawi
munthuyu wapezeka ndi nthendayi pachipatala china m'boma la Mzimba ndipo zotsatira zake zatsimikizika lolemba sabata ino ndi nthambi ya pabuliki hefe insichuti ofu Malawi
Female
Mlembiyu wati pakadali pano undunawu ukugwira ntchito ndi magulu ena okhudzidwa powunikira moyenera zankhaniyi
Mlembiyu wati pakadali pano undunawu ukugwira ntchito ndi magulu ena okhudzidwa powunikira moyenera zankhaniyi
Female
Nthenda ya Anthrax imayamba ndi kachilombo ka Bacteria kotchedwa Bacillus Anthracic ndipo kamakhudza nyama monga Ng'ombe, Mbuzi, Nkhumba komanso anthu
Nthenda ya Anfilakisi imayamba ndi kachilombo ka Bakiteliya kotchedwa Basilasi Anfilasiki ndipo kamakhudza nyama monga Ng'ombe, Mbuzi, Nkhumba komanso anthu
Female
Zina mwazizindikiro zanthendayi ndi zotupa zosapweteka zokhala ndi kanthu kakuda pakati pake, kupwanya mthupi, kukhosomola, kubanika popuma, kusanza komanso kutsekula m'mimba
Zina mwazizindikiro zanthendayi ndi zotupa zosapweteka zokhala ndi kanthu kakuda pakati pake, kupwanya mthupi, kukhosomola, kubanika popuma, kusanza komanso kutsekula m'mimba
Female
Bungwe lowona mtendere pa dziko lonse lotchedwa Heavenly Culture, World peace, Restoration of Light lapempha boma la Malawi kuti lithandize kulimbikitsa mtendere ndi mgwirizano
Bungwe lowona mtendere pa dziko lonse lotchedwa Hevenile kacha, waodi pisi, lisitoleshoni ofu laiti lapempha boma la Malawi kuti lithandize kulimbikitsa mtendere ndi mgwirizano
Female
mogwirizana ndi lamulo la dziko lonse lapansi. Mtsogoleri wa bungweli ku Malawi a Sphesihle Mdlalose omwe ndi nzika ya dziko la South Africa
mogwirizana ndi lamulo la dziko lonse lapansi. Mtsogoleri wa bungweli ku Malawi a Siphesile Mazyalose omwe ndi nzika ya dziko la saufi afilika
Female
anena izi lachitatu mu mzinda wa Lilongwe pamene bungweli lawo limalankhula ndi aphungu ena a nyumba ya malamulo pa nkhani yolengeza za mtendere ndi kutha kwa nkhondo
anena izi lachitatu mu mzinda wa Lilongwe pamene bungweli lawo limalankhula ndi aphungu ena a nyumba ya malamulo pa nkhani yolengeza za mtendere ndi kutha kwa nkhondo
Female
Polankhula ndi Angaliba, Madlalose adati cholinga cha bungwe lawo ndikufuna kulimbikitsa ntchito zamtendere padziko lonse lapansi potsatira malamulo a DPCW
Polankhula ndi Angaliba, Mazalose adati cholinga cha bungwe lawo ndikufuna kulimbikitsa ntchito zamtendere padziko lonse lapansi potsatira malamulo a Dipisi dabiliyu
Female
Tikuyesesa kugwira ntchito zothetsa nkhondo ndi kudzetsa mtendere Kwa anthu pa dziko lonse la pansi, anatero Madlalose
Tikuyesesa kugwira ntchito zothetsa nkhondo ndi kudzetsa mtendere Kwa anthu pa dziko lonse la pansi, anatero Mazalose
Female
Poyankhulapo wapampando wa bungwe loona za mtendere woyenera , ku nyumba ya malamulo Abel Kayembe, adati msonkhanowu ndi wothandiza kwambiri
Poyankhulapo wapampando wa bungwe loona za mtendere woyenera , ku nyumba ya malamulo Abelo Kayembe, adati msonkhanowu ndi wothandiza kwambiri
Female
moti udzathandizika kupereka ndondomeko yothana ndi gwero la mikangano ndi kupeza njira zokhazikika zothana ndi kusagwirizana
moti udzathandizika kupereka ndondomeko yothana ndi gwero la mikangano ndi kupeza njira zokhazikika zothana ndi kusagwirizana
Female
Ife aphunguwo tinadzipereka kale kulimbikitsa mtendere ndi bata m’dziko muno choncho izi zithandiza kuti ndondomeko ya mtendere ya dziko la 2017 ikwaniritsidwe, anatero a Kayembe
Ife aphunguwo tinadzipereka kale kulimbikitsa mtendere ndi bata m’dziko muno choncho izi zithandiza kuti ndondomeko ya mtendere ya dziko la twente seventini ikwaniritsidwe, anatero a Kayembe
Female
Bungwe la Heavenly Culture World Peace Restoration of Light likugwira ntchito yothana ndi nkhondo ndi nzika za maiko osiyana siyana kuphatikizapo South Africa ndi South Korea
Bungwe la hevenile kacha waodi pisi lisitoleshoni ofu laiti likugwira ntchito yothana ndi nkhondo ndi nzika za maiko osiyana siyana kuphatikizapo saufi afilika ndi Saufi koleya
Female
Mafumu a m'boma la mangochi ayamikila boma pa chitukuko cha nseu. Mafumu ochokera ku Mangochi ati ndiosangalala ndi chitukuko cha mseu wa Mangochi Makanjira
Mafumu a m'boma la mangochi ayamikila boma pa chitukuko cha nseu. Mafumu ochokera ku Mangochi ati ndiosangalala ndi chitukuko cha mseu wa Mangochi Makanjira
Female
Mafumuwa alankhula izi Lolemba lapitali pa msonkhano wa atolankhani omwe anakonza. Iwo ayamikira mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus Chakwera kamba koika chidwi pa mseu wu
Mafumuwa alankhula izi Lolemba lapitali pa msonkhano wa atolankhani omwe anakonza. Iwo ayamikira mtsogoleri wadziko lino Dokota Lazalasi Chakwera kamba koika chidwi pa mseu wu
Female
ndipo ati ndiokhutira ndizomwe boma likuchita. Padakali pano tikungodikira ndi chidwi kuyambika kwa ntchitoyi. Anatero mfumu yaikulu Makanjira omwe ndi imodzi mwa mafumu omwe analankhula
ndipo ati ndiokhutira ndizomwe boma likuchita. Padakali pano tikungodikira ndi chidwi kuyambika kwa ntchitoyi. Anatero mfumu yaikulu Makanjira omwe ndi imodzi mwa mafumu omwe analankhula
Female
Msonkhano wa atolankhaniwu unadza kutsatira mgwirizano wa makobidi ankhaninkhani okonzera nseu wu omwe mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus Chakwera anakasayinira ndi dziko la Saudi Arabia
Msonkhano wa atolankhaniwu unadza kutsatira mgwirizano wa makobidi ankhaninkhani okonzera nseu wu omwe mtsogoleri wadziko lino Dokota Lazalasi Chakwera anakasayinira ndi dziko la Saudi Alebiya
Female
Ku Mangochi moto wolusa watentha chipinda chosungilamo katundu pa sukulu ya sekondale ya Mangochi ndipo katundu wa ndalama zochuluka waonongeka
Ku Mangochi moto wolusa watentha chipinda chosungilamo katundu pa sukulu ya sekondale ya Mangochi ndipo katundu wa ndalama zochuluka waonongeka
Female
Olankhulila polisi ya Mangochi,Inspector Amina Tepani Daudi wauza Angaliba kuti ngoziyi yachitika usiku wathawu koma chomwe chinayambitsa motowo sichikudziwikabe
Olankhulila polisi ya Mangochi,Insipekita Amina Tepani Daudi wauza Angaliba kuti ngoziyi yachitika usiku wathawu koma chomwe chinayambitsa motowo sichikudziwikabe
Female
M'phunzitsi wamkulu pa sukuluyi, Amina Morris Gama anadziwa za ngoziyi pamene ophunzira ena anawadzutsa kunyumba kwawo, ophunzira ena olimba mtima
M'phunzitsi wamkulu pa sukuluyi, Amina Molisi Gama anadziwa za ngoziyi pamene ophunzira ena anawadzutsa kunyumba kwawo, ophunzira ena olimba mtima
Female
anayesera kuzimitsa motowo. Anatero Daudi. Padakali pano zadziwika kuti mabelo atatu a shuga, fridge, thumba lolemera 50 kilogalamu la mchere, mafuta ophikira
anayesera kuzimitsa motowo. Anatero Daudi. Padakali pano zadziwika kuti mabelo atatu a shuga, filiji, thumba lolemera fifite kilogalamu la mchere, mafuta ophikira
Female
matumba awiri a nyemba, malata ndi wina mwa katundu yemwe waonongeka. Mneneri wa apolisiyu wati Kuchuluka kwa ndalama za katundu yemwe wapsayu sikukudziwika
matumba awiri a nyemba, malata ndi wina mwa katundu yemwe waonongeka. Mneneri wa apolisiyu wati Kuchuluka kwa ndalama za katundu yemwe wapsayu sikukudziwika
Female
pomwe apolisi ali mkati kufufuzanso chomwe chinayambitsa motowu. Zonse zilimchimake kudikirira kulankhula kwa mtsogoleri wakale wa dziko lino Professor Peter Munthalika
pomwe apolisi ali mkati kufufuzanso chomwe chinayambitsa motowu. Zonse zilimchimake kudikirira kulankhula kwa mtsogoleri wakale wa dziko lino Pulofesa Pita Munthalika
Female
Ena mwa akulu akulu a chipani cha DPP omwe akuoneka pamalopa ndi monga a Geoge Chaponda, Francis Mphepo ,Bright Nsaka komaso Mary Navicha
Ena mwa akulu akulu a chipani cha Dipipi omwe akuoneka pamalopa ndi monga a Joji Chaponda, Fulansisi Mphepo ,Bulaiti Nsaka komaso Male Navicha
Female
Malingana ndi akulu akulu chipanichi akuti zina mwa zomwe alankhule ndi nkhani yokhudza kugwa kwa ndalama ya Malawi Kutsatira kugwa kwa mphamvu kwa ndalama ya Kwacha m'dziko muno ndi 44%
Malingana ndi akulu akulu chipanichi akuti zina mwa zomwe alankhule ndi nkhani yokhudza kugwa kwa ndalama ya Malawi Kutsatira kugwa kwa mphamvu kwa ndalama ya Kwacha m'dziko muno ndi fotefo pelesenti
Female
kampani yopanga zakumwa zozizilitsa kukhosi ya Coca Cola Beverages yakweza mitengo ya zakumwa zake kuyambira lero mdziko muno 16 November, 2023
kampani yopanga zakumwa zozizilitsa kukhosi ya kokakola bevelejezi yakweza mitengo ya zakumwa zake kuyambira lero mdziko muno sikisitini nivemba twente twente fili
Female
M'modzi mwa akuluakulu ku kampaniyi a Josephine Msaliwa ndiwo atsimikiza za izi kudzera mu chikalata chomwe atulutsa pa 15 November chaka chino
M'modzi mwa akuluakulu ku kampaniyi a Josofina Msaliwa ndiwo atsimikiza za izi kudzera mu chikalata chomwe atulutsa pa fifitini novemba chaka chino
Female
Pakadali pano Fanta azigulidwa pa mtengo wa K650 kuchoka pa K450 pamene Sobo Squash azigulidwa pa mtengo wa K6,000
Pakadali pano Fanta azigulidwa pa mtengo wa sikisi handede fifite kwacha kuchoka fo handede fifite kwacha pamene Sobo Sikwashi azigulidwa pa mtengo wa sikisi sauzande kwacha
Female
kuchoka pa K3, 700 pa malita awiri aliwonse. Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati dziko la Malawi
kuchoka pa fili sauzande seveni handede kwacha pa malita awiri aliwonse. Mtsogoleri wa dziko lino Dokota Lazalasi Chakwera wati dziko la Malawi
Female
lapeza mwai wa ngongole yokwana $174 million kuchoka ku IMF. Iwo ati kubwera kwa ndalamayi kuthandiza dziko la Malawi
lapeza mwai wa ngongole yokwana wani handiledi andi sevente fiolo miliyoni dolazi kuchoka ku aiemu efu. Iwo ati kubwera kwa ndalamayi kuthandiza dziko la Malawi
Female
pakuti dziko likwanitsa kugula feteleza ndi mankhwala mosavuta komanso kukonza mavuto ena monga njala
pakuti dziko likwanitsa kugula feteleza ndi mankhwala mosavuta komanso kukonza mavuto ena monga njala
Female
Iwo anati ndalamayinso ipindula kuti dziko liyambe kupanga zinthu zomagulitsa maiko ena chomcho ndalama za kunja sizidzisowa
Iwo anati ndalamayinso ipindula kuti dziko liyambe kupanga zinthu zomagulitsa maiko ena chomcho ndalama za kunja sizidzisowa
Female
Dr Chakwera anenanso kuti ayimitsa maulendo awo akunja mpaka chaka cha mawa pamodzi ndi maulendo a unduna ndi ogwira ntchito m'boma ndipo nduna zomwe zili kunja zione nsana wanjira
Dokota Chakwera anenanso kuti ayimitsa maulendo awo akunja mpaka chaka cha mawa pamodzi ndi maulendo a unduna ndi ogwira ntchito m'boma ndipo nduna zomwe zili kunja zione nsana wanjira
Female
Padakali pano atinso salola mikumano yachisawawa ya ogwira ntchito m'boma yomwe imatha kuononga ndalama. Pazakukweza mitengo mwachisawawa
Padakali pano atinso salola mikumano yachisawawa ya ogwira ntchito m'boma yomwe imatha kuononga ndalama. Pazakukweza mitengo mwachisawawa
Female
mtsogoleriyu wati unduna wa zamalonda uonetsetse kuti mitengo ya katundu siukukwezedwa mwachisawawa. Kwa ogwira ntchito ati unduna wa zachuma uwunike mlingo oyambira kulandira ndalama
mtsogoleriyu wati unduna wa zamalonda uonetsetse kuti mitengo ya katundu siukukwezedwa mwachisawawa. Kwa ogwira ntchito ati unduna wa zachuma uwunike mlingo oyambira kulandira ndalama
Female
komaso kwa ogwira ntchito m’boma akuyenera awakwezere ndalama ndikuunikanso mlingo odula misonkho. Pomaliza Dr Chakwera anati a Malawi ayembekezere zabwino ngakhale kuti adutsa mumzowawa
komaso Kwa ogwira ntchito m’boma akuyenera awakwezere ndalama ndikuunikanso mlingo odula misonkho. Pomaliza Dokota Chakwera anati a Malawi ayembekezere zabwino ngakhale kuti adutsa mumzowawa
Female
Koma anachenjeza kuti athana ndi aliense wofuna kubweza mmbuyo ntchito za boma kamba ka dyera
Koma anachenjeza kuti athana ndi aliense wofuna kubweza mmbuyo ntchito za boma kamba ka dyera
Female
Mtsogoleri wampingo wa Katolika padziko lonse lapansi Papa Francisco wasankha bambo Vincent Frederick Mwakhwawa kukhala bishopu othandiza (Auxiliary Bishop)
Mtsogoleri wampingo wa Katolika padziko lonse lapansi Papa Fulansisiko wasankha bambo Vinisenti Fulediliki Mwakhwawa kukhala bishopu othandiza (okuziliyale bishopu)
Female
wa Akidayosizi ya Lilongwe. Izi zalengezedwa ndi likulu lampingo pa dziko lonse ku Roma mu mzinda wa Vatican
wa Akidayosizi ya Lilongwe. Izi zalengezedwa ndi likulu lampingo pa dziko lonse ku Roma mu mzinda wa Vatikani
Female
Bambo Mwakhwawa asanasankhidwe kukhala bishopu osankhidwa othandiza, pomwe amatumikira mu Arkidayosizi ya Lilongwe ngati Vicar General
Bambo Mwakhwawa asanasankhidwe kukhala bishopu osankhidwa othandiza, pomwe amatumikira mu Akidayosizi ya Lilongwe ngati Vika Jenelo
Female
Wachitetezo wa mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika, Norman Chisale wamangidwa. Malinga ndi a polisi, a Chisale ali ndi ziwiri zitatu zoti akayankhe
Wachitetezo wa mtsogoleri wakale wa dziko lino a Pita Mutharika, Nomani Chisale wamangidwa. Malinga ndi a polisi, a Chisale ali ndi ziwiri zitatu zoti akayankhe
Female
Pakadali pano a Chisale ali ku polisi ya Lingadzi komwe awauze mlandu omwe apalamula. Koma malinga ndi malipoti, ndi nkhani zokhudzana ndi zomwe adayankhula pa kanema wina mdziko muno masiku apitawa
Pakadali pano a Chisale ali ku polisi ya Lingadzi komwe awauze mlandu omwe apalamula. Koma malinga ndi malipoti, ndi nkhani zokhudzana ndi zomwe adayankhula pa kanema wina mdziko muno masiku apitawa
Female
Boma kudzera mu unduna wake wa zachuma wati laika ndondomeko zofuna kuchepetsa mavuto kutsatira kugwa mphanvu kwa ndalama ya kwacha
Boma kudzera mu unduna wake wa zachuma wati laika ndondomeko zofuna kuchepetsa mavuto kutsatira kugwa mphanvu kwa ndalama ya kwacha
Female
Izi zanenedwa ndi nduna muundunau a Simplex Chithyola Banda ku Bingu International Convention Centre mu mzinda wa Lilongwe kudzera pa msonkhano wa atolankhani
Izi zanenedwa ndi nduna muundunau a Simpulekisi Chithyola Banda ku Bingu intaneshono konveshono senta mu mzinda wa Lilongwe kudzera pa msonkhano wa atolankhani
Female
Zina mwa izo boma liyamba kupereka ndalama yokwana K50,000 pamwezi kwa anthu ocholera mabanja 184,920 omwe anakhudzika ndi Cyclone freddy mmaboma 9
Zina mwa izo boma liyamba kupereka ndalama yokwana fifite sauzande kwacha pamwezi kwa anthu ocholera mabanja wani handede andi eite folo sauzande naini handede andi twente omwe anakhudzika ndi saikuloni fulede mmaboma naini
Female
Bomalinso lakweza chiwerengero cha anthu olandira mtukula pakhomo kuchoka 2 million kufika 3 million
Bomalinso lakweza chiwerengero cha anthu olandira mtukula pakhomo kuchoka thu miliyoni kufika fili miliyoni
Female
Laikanso ndondomeko yoika pa mtukula pakhomo anthu ammatauni mabanja okwana 105 thousand, 105 thousand omwe azilandira K150,000 pa mwezi
Laikanso ndondomeko yoika pa mtukula pakhomo anthu ammatauni mabanja okwana wani handede andi faifi sauzande, wani handede andi faifi sauzande omwe azilandira wani handede andi fifite sauzande kwacha pa mwezi
Female
Pa nkhani ya ntchito ndunayi yati akukambirana ndi mabungwe owona za ntchito kuti akweze malipilo. Ananenaso kuti boma lilemba azachipatala okwana 2741
Pa nkhani ya ntchito ndunayi yati akukambirana ndi mabungwe owona za ntchito kuti akweze malipilo. Ananenaso kuti boma lilemba azachipatala okwana thu sauzande seveni handede andi fote wani
Female
ndiponso likulumikizana ndi maiko ena kuti boma lizitumiza anthu pafupifupi 5000 kukagwira ntchito kunja. A Chithyola Banda anachenjezanso kuti boma lakhwimitsa chitetezo pamalonda a ndalama za kunja
ndiponso likulumikizana ndi maiko ena kuti boma lizitumiza anthu pafupifupi faifi sauzande kukagwira ntchito kunja. A Chithyola Banda anachenjezanso kuti boma lakhwimitsa chitetezo pamalonda a ndalama za kunja
Female
ndipo likwidzinga aliyese ochita malonda a ndalama za kunja mosatsata malamulo. Msonkhano wa atolankhaniwu umene sunapereke mwai kwa atolankhani kufusa mafunso
ndipo likwidzinga aliyese ochita malonda a ndalama za kunja mosatsata malamulo. Msonkhano wa atolankhaniwu umene sunapereke mwai kwa atolankhani kufusa mafunso
Female
unadza kutsatira kugwa mphanvu kwa ndalama ya Malawi sabata yapitayi ndi 44 percent. Kugwa kwandalamaku kwapangitsa kuti zinthu zambiri zikwere mitengo
unadza kutsatira kugwa mphanvu kwa ndalama ya Malawi sabata yapitayi ndi fotefo pelesenti. Kugwa kwandalamaku kwapangitsa kuti zinthu zambiri zikwere mitengo
Female
Komabe boma linati ngati njira yothana ndi mavuto azachuma njira yabwino inali kugwetsa mphanvu ya ndalamayi ndipo anatsimikiza kuti posachedwapa zinthu ziyenda bwino
Komabe boma linati ngati njira yothana ndi mavuto azachuma njira yabwino inali kugwetsa mphanvu ya ndalamayi ndipo anatsimikiza kuti posachedwapa zinthu ziyenda bwino
Female
Ngati njila imodzi yopitisila patsogolo mtendele komaso mgwilizano pakati pa asilamu komaso azipembezo Zina, wapampando wa Qadria Muslim association of Malawi mchigawo chakummawa
Ngati njila imodzi yopitisila patsogolo mtendele komaso mgwilizano pakati pa asilamu komaso azipembezo Zina, wapampando wa kwadiliya muzilimu asosiyeshoni ofu Malawi mchigawo chakummawa
Female
Shelkh Haj Balasan anakonza msonkhano loweluka pa 11 November 2023 mmudzi mwa Mpasuka mfumu yaikulu Nkula m'boma la Machinga
Shekhi Haji Balasani anakonza msonkhano loweluka pa leveni Novemba twente twente fili mmudzi mwa Mpasuka mfumu yaikulu Nkula m'boma la Machinga
Female
ndicholinga chofuna kuyanjanisa mbali ziwiri zomwe panali kusanvana pankhani yokhuza umwini wa mzikiti
ndicholinga chofuna kuyanjanisa mbali ziwiri zomwe panali kusanvana pankhani yokhuza umwini wa mzikiti
Female
Mwambo omwe unalemekezedwa ndi wapampando wa bungwe la Qadria Muslim Association of Malawi shelkh Jafar Kawinga omwenso anali mlendo olemekezeka
Mwambo omwe unalemekezedwa ndi wapampando wa bungwe la kwadiliya muzilimu asosiyeshoni ofu Malawi shekhi Jafa Kawinga omwenso anali mlendo olemekezeka
Female
wapampando wa bungweli mchigawo chakummwela a Ar hajji mussa , Mufti dinala ochokera Kwa chamba, Mfti sayeed kuchokera ku zomba , shelkh kavina, mafumu kungotchulapo ochepa chabe
wapampando wa bungweli mchigawo chakummwela a A haji mussa , Mufuti dinala ochokera Kwa chamba, Mufuti sayidi kuchokera ku zomba , shekhi kavina, mafumu kungotchulapo ochepa chabe
Female
Mmawu awo a Jafar Kawinga ngati membala wa Pablic Affair Committe (PAC) anati asilamu tikhale oyamba kubwelesa mtendele
Mmawu awo a Jafa Kawinga ngati membala wa pabuliki afeya komiti (PAKI) anati asilamu tikhale oyamba kubwelesa mtendele
Female
ngati mmene aneneli anthu osiyanasiyan amachitila kupatula kusiyana zikhulupiliro komaso ziphunzitso koma tili ndi udindo owonesesa kuti pakati pathu Pali kulumikizana
ngati mmene aneneli anthu osiyanasiyan amachitila kupatula kusiyana zikhulupiliro komaso ziphunzitso koma tili ndi udindo owonesesa kuti pakati pathu Pali kulumikizana
Female
zomwe zichitiseso kuti anthu azipembezo Zina athe kukhumbila chipembezo chathu ndikulowanso kumene koma tikakhala amitima yosayanjana ngati mulungu sangakondwe
zomwe zichitiseso kuti anthu azipembezo Zina athe kukhumbila chipembezo chathu ndikulowanso kumene koma tikakhala amitima yosayanjana ngati mulungu sangakondwe
Female
Iwo analonjezaso kuonesesa kuti pa utsogoleri wawo awonesesa kuti ana achisilam akukhala ophunzila bwino mbali zonse maphunzilo achisilamu ngati madrassa komaso maphunzilo achikunja
Iwo analonjezaso kuonesesa kuti pa utsogoleri wawo awonesesa kuti ana achisilamu akukhala ophunzila bwino mbali zonse maphunzilo achisilamu ngati madilasa komaso maphunzilo achikunja
Female
Mwambo omwe unayambika pambuyo pa pemphero la dhuhur unasangalasidwa ndi azimayi achisilamu omwe anazafika pa malowa ndi nyimbo zao zosiyanasiyana zotamanda mtumiki Muhammad komaso mulungu
Mwambo omwe unayambika pambuyo pa pemphero la duhula unasangalasidwa ndi azimayi achisilamu omwe anazafika pa malowa ndi nyimbo zao zosiyanasiyana zotamanda mtumiki Muhamadi komaso mulungu
Female
Mtsogoleri wa bungwe la Football Association of Malawi, Walter Nyamilandu Manda wamema mtundu wa a Malawi kuti apikisana nawo pampando wa utsogoleri wa bungweli pa 16 December 2023
Mtsogoleri wa bungwe la futubo asosiyeshoni ofu Malawi, Wota Nyamilandu Manda wamema mtundu wa a Malawi kuti apikisana nawo pampando wa utsogoleri wa bungweli pa sikisitini Disemba twente twente fili
Female
Poyankhula pa msonkhano wa atolankhani, mu mzinda wa Blantyre, Nyamilandu wati wapanga chisankhochi chifukwa akufuna apitilize zitukuko zomwe anaziyamba komaso kupitisa patsogolo mpira wamiyendo mudziko muno
Poyankhula pa msonkhano wa atolankhani, mu mzinda wa Bulantaya, Nyamilandu wati wapanga chisankhochi chifukwa akufuna apitilize zitukuko zomwe anaziyamba komaso kupitisa patsogolo mpira wamiyendo mudziko muno
Female
Iye anapitiliza kunena kuti akasankhidwanso kukhala mtsogoleri wa bungweli ntchito za mpira zipita chitsogolo, koma ngati a Malawi atasankhe munthu wina yemwe sakudziwika komwe akuchokera
Iye anapitiliza kunena kuti akasankhidwanso kukhala mtsogoleri wa bungweli ntchito za mpira zipita chitsogolo, koma ngati a Malawi atasankhe munthu wina yemwe sakudziwika komwe akuchokera
Female
koma akufuna kuphunzila za utsogoleriwu, chitukuko sichitheka. Pakadali pano ntchito yokopa anthu popikisana utsogoleri wa mpandowu Ili nkati
koma akufuna kuphunzila za utsogoleriwu, chitukuko sichitheka. Pakadali pano ntchito yokopa anthu popikisana utsogoleri wa mpandowu Ili nkati
Female
ndipo Nyamilandu wati fundo yake ndiyotchedwa bridging the gap. Bwalo la milandu lalikulu ku Lilongwe lakana pempho la belo a Lester Maganga
ndipo Nyamilandu wati fundo yake ndiyotchedwa bulijing’i ve gapu. Bwalo la milandu lalikulu ku Lilongwe lakana pempho la belo a Lesita Maganga
Female
yemwe akumuganizira mlandu woti anapha Allan Witika yemwe amagwira ntchito ku kampani ya Coca Cola. Oweruza milandu kubwaloli a Mzondi Mvula
yemwe akumuganizira mlandu woti anapha Alani Witika yemwe amagwira ntchito ku kampani ya kokakola. Oweruza milandu kubwaloli a Mzondi Mvula
Female
ndiwo apeleka chigamulochi. A banja la Wittika a Willy Zingati , adati iwo achilandira chigamulochi ndipo ayembekeza chilungamo pa nkhaniyi
ndiwo apeleka chigamulochi. A banja la Wittika a Wile Zingati , adati iwo achilandira chigamulochi ndipo ayembekeza chilungamo pa nkhaniyi
Female
A Allan Wittika anapezeka atafa ku area 15 mu mzinda wa Lilongwe pa 20 September chaka chino. Banki yaikulu mdziko muno ya Reserve
A Alani Wittika anapezeka atafa ku eliya fifitini mu mzinda wa Lilongwe pa twente sepitemba chaka chino. Banki yaikulu mdziko muno ya lizevu
Female
yachepetsa mphanvu ya ndalama ya Malawi ya kwacha yomwe imagulidwa pa 1180 kufika pa 1700
yachepetsa mphanvu ya ndalama ya Malawi ya kwacha yomwe imagulidwa pa wani sauzande wani handede andi eite kufika pa wani sauzande seveni handede
Female
Ndalamayi yagwa mphanvu pafupifupi ndi 44 percent. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe Bankiyi yatulutsa ndipo ziyambika pa 9 November 2023
Ndalamayi yagwa mphanvu pafupifupi ndi fotefo pelesenti. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe Bankiyi yatulutsa ndipo ziyambika pa naini novemba twente twente fili
Female