audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
Ngati njira imodzi yopititsa patsogolo ntchito yopereka madzi aukhondo m'boma la Mangochi bungwe lotchedwa Evedence Action likugwira ntchito yoika mankhwala a Chlorine mmijingo | Ngati njira imodzi yopititsa patsogolo ntchito yopereka madzi aukhondo m'boma la Mangochi bungwe lotchedwa evidensi akishoni likugwira ntchito yoika mankhwala a kulolini mmijingo | Female | |
Poyendera ntchitoyi mdera la Namiyasi lowelukali wachiwiri wa nduna ya zaumoyo Halima Daudi wayamikira ntchitoyi kunena kuti ikuthandiza kulimbana ndi matenda otsekula mmimba omwe amavuta m'bomali | Poyendera ntchitoyi mdera la Namiyasi lowelukali wachiwiri wa nduna ya zaumoyo Halima Daudi wayamikira ntchitoyi kunena kuti ikuthandiza kulimbana ndi matenda otsekula mmimba omwe amavuta m'bomali | Female | |
Polankhula ndi Angaliba Daudi anati izi zikuthandiza kuti anthu azimwa madzi otetezeka zomwe zipititse patsogolo thanzi lao | Polankhula ndi Angaliba Daudi anati izi zikuthandiza kuti anthu azimwa madzi otetezeka zomwe zipititse patsogolo thanzi lao | Female | |
Mmodzi mwa anthu omwe akupindula ndi ntchitoyi Magret Ajidu anathokoza adindo powaganizira ndi ndondomekoyi yomwe anati ikupindulila anthu ochuluka omwe amagwiritsa ntchito mijigo | Mmodzi mwa anthu omwe akupindula ndi ntchitoyi Magileti Ajidu anathokoza adindo powaganizira ndi ndondomekoyi yomwe anati ikupindulila anthu ochuluka omwe amagwiritsa ntchito mijigo | Female | |
Padakali pano Evidence Action ikugwira ntchitoyi mmaboma 8 mdziko muno ndipo bungweri lakwanitsa kale kuika makina otulutsa chlorine opitilila 16,000 | Padakali pano evidensi akishoni ikugwira ntchitoyi mmaboma eiti mdziko muno ndipo bungweri lakwanitsa kale kuika makina otulutsa kulolini opitilila sikisitini sauzande | Female | |
Bwalo laling'ono lamilandu la Dalton mu mzinda wa Blantyre latsimikiza za tsiku lolemba pa 6 November kuti ndi pomwe lidzapeleke chigamulo pa nkhani ya bambo Suez Chilombo | Bwalo laling'ono lamilandu la Datoni mu mzinda wa Bulantaya latsimikiza za tsiku lolemba pa sikisi novemba kuti ndi pomwe lidzapeleke chigamulo pa nkhani ya bambo Suwezi Chilombo | Female | |
omwe akuwaganizila kuti anagwirira mwana wawo wamkazi womupeza. Mlanduwu omwe wakhala ukukambidwa kuchokera mchaka cha 2020 | omwe akuwaganizila kuti anagwirira mwana wawo wamkazi womupeza. Mlanduwu omwe wakhala ukukambidwa kuchokera mchaka cha twente twente | Female | |
pomwe akuganizila kuti ndi nthawi yomwe bamboyu anachita izi, tsopano wafika kumapeto komva mbali za mboni zonse zokhudzidwa kuphatikizapo a katswiri a chipatala komwe anakamuyeza mtsikanayu kuti atsimikize za nkhaniyi | pomwe akuganizila kuti ndi nthawi yomwe bamboyu anachita izi, tsopano wafika kumapeto komva mbali za mboni zonse zokhudzidwa kuphatikizapo a katswiri a chipatala komwe anakamuyeza mtsikanayu kuti atsimikize za nkhaniyi | Female | |
Nkulu omenyela ana ufulu ku bungwe la Forum for Youth and Women Empowerment, omwenso ndi amene akhala akuchita chotheka kuti nkhaniyi ikambidwe ku bwalo la milandu mpaka pamapeto | Nkulu omenyela ana ufulu ku bungwe la folamu fo yufi andi wimeni impawamenti , omwenso ndi amene akhala akuchita chotheka kuti nkhaniyi ikambidwe ku bwalo la milandu mpaka pamapeto | Female | |
Steve Belson wati iwo akudikila ndi chidwi kufuna kuona chilungamo cha nkhaniyi mmene chiyendere. Bambo Suez Chilombo akuwaganizila kuti anagwirira mwana wawoyu | Steve Beosoni wati iwo akudikila ndi chidwi kufuna kuona chilungamo cha nkhaniyi mmene chiyendere. Bambo Suwezi Chilombo akuwaganizila kuti anagwirira mwana wawoyu | Female | |
yemwe nthawi imeneyo anali ndi zaka 12 zakubadwa, ndipo yemwe akuwaimila pa mlandu a Chilombo, Fostino Maere | yemwe nthawi imeneyo anali ndi zaka thwelofu zakubadwa, ndipo yemwe akuwaimila pa mlandu a Chilombo, Fositino Maere | Female | |
anakana zoti mtsikanayu anagwiriridwa ponena kuti umboni wa chipatala sukutsimikiza zenizeni zoonetsa kuti kugwirira kunachitikadi kapena ayi | anakana zoti mtsikanayu anagwiriridwa ponena kuti umboni wa chipatala sukutsimikiza zenizeni zoonetsa kuti kugwirira kunachitikadi kapena ayi | Female | |
Ku Mangochi a police apa Makokola amanga sing'anga wina wa zaka 20 zakubadwa pa mlandu oganiziridwa kuti anagwiririra msungwana wa zaka 13 pomwe amagwira ntchito yake | Ku Mangochi a polisi apa Makokola amanga sing'anga wina wa zaka twente zakubadwa pa mlandu oganiziridwa kuti anagwiririra msungwana wa zaka fetini pomwe amagwira ntchito yake | Female | |
Mneneri wa a police ya Mangochi Inspector Amina Tepani Daudi watsimikiza za izi ndipo wati zinachitika mmudzi mwa Mpemba 2. Malingana ndi Daudi ,Makolo a msungwanayu | Mneneri wa a polisi ya Mangochi Insipekita Amina Tepani Daudi watsimikiza za izi ndipo wati zinachitika mmudzi mwa Mpemba thu. Malingana ndi Daudi ,Makolo a msungwanayu | Female | |
anaitana Simoni amene amakhala moyandikana kamba ka vuto la mmimba momwe mtsikanayu wakhala akudandaula,ndipo adapereka thandizo lake la mankhwala | anaitana Simoni amene amakhala moyandikana kamba ka vuto la mmimba momwe mtsikanayu wakhala akudandaula,ndipo adapereka thandizo lake la mankhwala | Female | |
Pa 31 October Simon anauza mtsikanayu kuti akatengenso mankhwala ena komano kunyumba yake komwe anakamugwiririra | Pa fetewani okutoba Simoni anauza mtsikanayu kuti akatengenso mankhwala ena komano kunyumba yake komwe anakamugwiririra | Female | |
Mwanayo anatsinakhutu Makolo ake omwe nao sanaikhalile nkhaniyo koma kukanena ku police.Chipatala cha Koche chinatsimikiza kuti msungwanayu anagwiriridwadi | Mwanayo anatsinakhutu Makolo ake omwe nao sanaikhalile nkhaniyo koma kukanena ku polisi.Chipatala cha Koche chinatsimikiza kuti msungwanayu anagwiriridwadi | Female | |
Padakali pano apolisiwa ati Simon akalowa kukhothi posachedwa kukayankha mlandu ogonana ndi mwana wachichepere Simoniyu amachokera mmudzi mwa Sandika mfumu yaikulu Mlumbe m'boma la Zomba | Padakali pano apolisiwa ati Simoni akalowa kukhothi posachedwa kukayankha mlandu ogonana ndi mwana wachichepere Simoniyu amachokera mmudzi mwa Sandika mfumu yaikulu Mlumbe m'boma la Zomba | Female | |
Team ya Mighty Mukuru Wanderers yapitilira mu mpikitsano wa pachema FDH bank. Wanderers yapitiliza pomwe inasiila sabata latha mumpikisano wa TNM | Timu ya Maite Mukuru Wandilazi yapitilira mu mpikitsano wa pachema efudietchi banki. Wandilazi yapitiliza pomwe inasiila sabata latha mumpikisano wa Tieniemu | Female | |
pomwe inafananiza mphamvu ndi team ya Nyasa Big Bullets . Zigoli za F.Mkonda ,Vincent nyangulu,Vitumbiko kumwenda ndi lsaac chair kaliat | pomwe inafananiza mphamvu ndi team ya Nyasa Bigi buletsi . Zigoli za efu.Mkonda ,Vinisenti nyangulu,Vitumbiko kumwenda ndi aizeki Tcheya kaliat | Female | |
zathandiza team ya noma kut ipambane 4-1 pabwalo la zamasewero la kamuzu. Chigoli cha KB chinachokera Kwa Zeriat Nkhoma kuzera pa penalty | zathandiza timu ya noma kut ipambane folo-wani pabwalo la zamasewero la kamuzu. Chigoli cha keyibi chinachokera Kwa Zeliyati Nkhoma kuzera pa penate | Female | |
Pamasewero ena team ya Big bullets yagonjesa team ya Chitipa united pa bwalo la Rumphi ndi zigoli ziwiri Kwa duu zomwe anamwesa ndi Babatunde komanso Anthony Mfune | Pamasewero ena team ya Big Bullets yagonjesa timu ya Chitipa yunaitedi pa bwalo la Rumphi ndi zigoli ziwiri Kwa duu zomwe anamwesa ndi Babatunde komanso Antone Mfune | Female | |
M'mene zatelemu team ya Noma ikumana ndi Nyasa Big bullets mundime ya semifinals. Masewero ena amundime ya ma team 8 iliko mawa | M'mene zatelemu timu ya Noma ikumana ndi Nyasa Bigi buletsi mundime ya semifainozi. Masewero ena amundime ya ma timu eiti iliko mawa | Female | |
pamene Nyasa Big bullets reserve ikumana ndi team ya Blue Eagles pabwaro la kamuzu ndipo team ya extreme fc ikumana ndi team ya changalume barracks pa bwalo la Balaka | pamene Nyasa bigi buletsi lizevu ikumana ndi team ya Bulu igozi pabwaro la kamuzu ndipo timu ya ekisitilimu efisi ikumana ndi timu ya changalume balakisi pa bwalo la Balaka | Female | |
Bungwe la ZICO Forward lati lipitiliza kugwira ntchito zake m’madera ochuluka mdzikomuno. Izi zalankhulidwa pamwambo waukwati wa chifumu omwe unachitika loweluka pa 13 August 2022 | Bungwe la ZIKO Folowadi lati lipitiliza kugwira ntchito zake m’madera ochuluka mdzikomuno. Izi zalankhulidwa pamwambo waukwati wa chifumu omwe unachitika loweluka pa fetini ogasiti twente twente thu | Female | |
m'mudzi mwa mfumu yaikulu kadewele, mdera la mfumu yaing'ono Robin. Polankhula pa mwambo wopelekeza mfumu yaing'ono James yomwe yatenga Janet kukhala mkazi wake | m'mudzi mwa mfumu yaikulu kadewele, mdera la mfumu yaing'ono Robini. Polankhula pa mwambo wopelekeza mfumu yaing'ono Jamusi yomwe yatenga Janeti kukhala mkazi wake | Female | |
Owen Odinga Chitsulo yemwe ndi National cordinator wabungweli wati cholinga chawo ndichofuna kuthandiza azimayi amasiye ndi anthu okalamba | Oweni Odinga Chitsulo yemwe ndi Neshono kodineta wabungweli wati cholinga chawo ndichofuna kuthandiza azimayi amasiye ndi anthu okalamba | Female | |
Bungwe la ZICO Forward likugwira ntchito zake pansi pa bungwe lomwe likutchedwa zizi Community foundation for women's Relief Advancement and Development ndipo likugwiranso ntchito limodzi ndi bungwe la Angaliba foundation | Bungwe la ZIKO Folowadi likugwira ntchito zake pansi pa bungwe lomwe likutchedwa zizi komyunite faundeshoni fo wimenzi lilifi adivansimenti andi divelopumenti ndipo likugwiranso ntchito limodzi ndi bungwe la Angaliba faundeshoni | Female | |
Pa mwambowu kunalinso anthu ochuluka omwe ndikuphatikizapo mafumu akulu akulu monga T/A Kadewele komanso T/A Ntchema omwe ndiochokera mb'oma la Chiradzulu | Pa mwambowu kunalinso anthu ochuluka omwe ndikuphatikizapo mafumu akulu akulu monga tie Kadewele komanso Tie Ntchema omwe ndiochokera mb'oma la Chiradzulu | Female | |
Kupatula kudya ndikumwelera pa tsiku la ukwatili, bungweli linalimbikitsanso anthu za kufunika kothamangira kuchipatala nsanga ngati apezeka ndi vuto la fistula | Kupatula kudya ndikumwelera pa tsiku la ukwatili, bungweli linalimbikitsanso anthu za kufunika kothamangira kuchipatala nsanga ngati apezeka ndi vuto la fisichula | Female | |
Mnyamata wina oyimba Nyimbo za Amapiano waitanidwa kukaimba ku Show ya Kizz Daniel atayesa Mwayi. Masiku apitawo Mnyamata otchedwa Biggie Lu | Mnyamata wina oyimba Nyimbo za Amapiano waitanidwa kukaimba ku Sho ya Kizi Daniele atayesa Mwayi. Masiku apitawo Mnyamata otchedwa Bigi Lu | Female | |
yemwe amayimba chamba Cha Amapiano Ku Malawi wapeza Mwayi okayimba nawo ku msangalutso wamaimbidwe ku mzinda wa Lilongwe pa 27 August ku Golf Club | yemwe amayimba chamba Cha Amapiano Ku Malawi wapeza Mwayi okayimba nawo ku msangalutso wamaimbidwe ku mzinda wa Lilongwe pa twente seveni ogasiti ku gofu kilabu | Female | |
Mu kanema amene Biggie Lu akuoneka akuzifotokoza yekha kuti ndikatswiri kwambiri ndipo anafotokoza ndi mtima onse kuti iyeyo ndi mchochombe pa nkhani yosangalasa Anthu pa Stage | Mu kanema amene Bigi Lu akuoneka akuzifotokoza yekha kuti ndikatswiri kwambiri ndipo anafotokoza ndi mtima onse kuti iyeyo ndi mchochombe pa nkhani yosangalasa Anthu pa Siteji | Female | |
Yollam Kawanga amene Ali mkulu ndi mtsogoleri wa Epic Lifestyle imene ikubwelesa Kizz Daniel ataona izi adakapanga comment kuvomereza kuti Biggie Lu ayembekeze kuitchailidwa lamya ndipo zidathekadi | Yolamu Kawanga amene Ali mkulu ndi mtsogoleri wa Epiki laifisitayilo imene ikubwelesa Kizi Daniele ataona izi adakapanga komenti kuvomereza kuti Bigu Lu ayembekeze kuitchailidwa lamya ndipo zidathekadi | Female | |
Pamene Angaliba itamufikila Biggie Lu kumufusa iye adati ndiokondwa ndipo ali okonzeka kukasangalasa. Nyimbo Zina zomwe adayimba ndi monga Vuto ndi Amapiano, No Mwayi | Pamene Angaliba itamufikila Bigi Lu kumufusa iye adati ndiokondwa ndipo ali okonzeka kukasangalasa. Nyimbo Zina zomwe adayimba ndi monga Vuto ndi Amapiano, No Mwayi | Female | |
Phungu wa nyumba ya malamulo wa Ntchisi North East Olipa Chimangeni wapepha nduna ya za umoyo kuti aganizile zokulitsa chipatala cha ching'ono cha Thondo kukhala chipatala chachikulu | Phungu wa nyumba ya malamulo wa Ntchisi Nofi isiti Olipa Chimangeni wapepha nduna ya za umoyo kuti aganizile zokulitsa chipatala cha ching'ono cha Thondo kukhala chipatala chachikulu | Female | |
poganizila kuti chipatala cha Ntchisi chomwe amatumizilako chili kutali ndi madera ena mbali ya boma la Ntchisi. Achimangeni amayankhula izi mnyumba ya malamulo | poganizila kuti chipatala cha Ntchisi chomwe amatumizilako chili kutali ndi madera ena mbali ya boma la Ntchisi. Achimangeni amayankhula izi mnyumba ya malamulo | Female | |
pomwe anduna a za umoyo amayankha mafuso kuchokera Kwa aphungu osiyanasiyana. Achimangeni anatiso boma kudzera ku unduna wa za umoyo uganizilenso zokulitsa zipatala za Ndinda ndi Msambakusi | pomwe anduna a za umoyo amayankha mafuso kuchokera Kwa aphungu osiyanasiyana. Achimangeni anatiso boma kudzera ku unduna wa za umoyo uganizilenso zokulitsa zipatala za Ndinda ndi Msambakusi | Female | |
malingana ndi kuti chiwerengero cha anthu chikukwera pafupipafupi zomwe zikupangitsa kuti zipatala zambili mu zidzadza, kotero pamakhala povuta kuthandiza anthu | malingana ndi kuti chiwerengero cha anthu chikukwera pafupipafupi zomwe zikupangitsa kuti zipatala zambili mu zidzadza, kotero pamakhala povuta kuthandiza anthu | Female | |
Phunguyu anapitiliza kunena kuti azimayi oyembekezera akuvutika kwambiri mu thawi yochila maka chifukwa cha mitunda italiitali, komanso thawi ya mvula mayendedwe amavuta | Phunguyu anapitiliza kunena kuti azimayi oyembekezera akuvutika kwambiri mu thawi yochila maka chifukwa cha mitunda italiitali, komanso thawi ya mvula mayendedwe amavuta | Female | |
Koma poyankhapo wachiwiri kwa nduna ya za umoyo Enock Phale anati za mavuto amenewo akudziwa bwino zikungofunika kuti a Chimangeni alembere kalata ku unduna wa za umoyo kuti athandizidwe moyenera | Koma poyankhapo wachiwiri kwa nduna ya za umoyo Enoki Phale anati za mavuto amenewo akudziwa bwino zikungofunika kuti a Chimangeni alembere kalata ku unduna wa za umoyo kuti athandizidwe moyenera | Female | |
koma boma ndi lokozeka kutengapo mbali pofuna kusamalila anthu onse mdziko muno chifukwa choti ndi boma lokomera onse | koma boma ndi lokozeka kutengapo mbali pofuna kusamalila anthu onse mdziko muno chifukwa choti ndi boma lokomera onse | Female | |
Phungu wanyumba ya malamulo wa dera la ku M'mawa kwa boma la Chikwawa a Ilias Callim wati pano ndi wokondwa kuti tsopano m'boma la chikwawa mwafika madzi a mmipopi | Phungu wanyumba ya malamulo wa dera la ku M'mawa kwa boma la Chikwawa a Iliyasi kalimu wati pano ndi wokondwa kuti tsopano m'boma la chikwawa mwafika madzi a mmipopi | Female | |
A Callim ati ngakhale kuti anavutika ndi ngozi zogwa mwadzidzi monga Gombe Ana zomwe zinapangitsa kuti madzi akhale ovuta koma pano wati anthu aku chikwawa ndi wokondwa tsopano kuti akumwa madzi abwino | A kalimu ati ngakhale kuti anavutika ndi ngozi zogwa mwadzidzi monga Gombe Ana zomwe zinapangitsa kuti madzi akhale ovuta koma pano wati anthu aku chikwawa ndi wokondwa tsopano kuti akumwa madzi abwino | Female | |
Iye wayamikila Boma kudzera ku unduna wa za madzi pobweretsa madzi abwino, ndipo anapitiliza kunena kuti ngakhale madera ena sanafike koma iye ali ndi chikhulupiliro kuti madziwa afikila madera ena | Iye wayamikila Boma kudzera ku unduna wa za madzi pobweretsa madzi abwino, ndipo anapitiliza kunena kuti ngakhale madera ena sanafike koma iye ali ndi chikhulupiliro kuti madziwa afikila madera ena | Female | |
Callim anatinso pano akuyankhula ndi mabungwe ena komanso anthu akufuna kwabwino kuti atengepo mbali pobweretsa madzi mbali zina za boma la chikwawa | Kalimu anatinso pano akuyankhula ndi mabungwe ena komanso anthu akufuna kwabwino kuti atengepo mbali pobweretsa madzi mbali zina za boma la chikwawa | Female | |
ndipo akukhulupilira kuti izi zitheka chifukwa chifukwa anthu amabungwe ena anabwera kale ndi zitukuko zina. Callim ndi phungu wanyumba ya malamulo wa dela la Ku Mmawa kwa Boma la Chikwawa | ndipo akukhulupilira kuti izi zitheka chifukwa chifukwa anthu amabungwe ena anabwera kale ndi zitukuko zina. Kalimu ndi phungu wanyumba ya malamulo wa dela la Ku Mmawa kwa Boma la Chikwawa | Female | |
Pamene zokambirana za aphungu anyumba ya malamulo zikupitilira ku nyumba ya malamulo mu mzinda wa Lilongwe, Phungu wa dera la Mangochi West a Reuben Kanyama anauza a nduna a zamagetsi a Ibrahim Matola | Pamene zokambirana za aphungu anyumba ya malamulo zikupitilira ku nyumba ya malamulo mu mzinda wa Lilongwe, Phungu wa dera la Mangochi Wesiti a Rubeni Kanyama anauza a nduna a zamagetsi a Ibulahimu Matola | Female | |
kuti vuto la kuonongeka kwa ma transformer ku Mangochi west kukuwasokoneza ntchito zamalonda zomwe zaimilatu pakadalipano. Phunguyu ananena izi kwa nduna ya zamagetsi mnyumbayi | kuti vuto la kuonongeka kwa ma thilansifoma ku Mangochi wesiti kukuwasokoneza ntchito zamalonda zomwe zaimilatu pakadalipano. Phunguyu ananena izi kwa nduna ya zamagetsi mnyumbayi | Female | |
pamene aphungu amapatsidwa mwayi wofusa mafuso nduna zokhudzidwa. koma poyankhula ndi Angaliba online Kanyama anati dera lakwao anthu akuvutika ndi magetsi | pamene aphungu amapatsidwa mwayi wofusa mafuso nduna zokhudzidwa. koma poyankhula ndi Angaliba onilaini Kanyama anati dera lakwao anthu akuvutika ndi magetsi | Female | |
ndipo iye wakhala akupempha kwa zaka ziwiri tsopano mnyumbayi, maka anthu omwe amapanga ma business ootchelera, ometa, azigayo komaso asaluni kungotchulako ochepa, zomwe zimathandiza anthu akumudzi ambiri | ndipo iye wakhala akupempha kwa zaka ziwiri tsopano mnyumbayi, maka anthu omwe amapanga ma buzinesi ootchelera, ometa, azigayo komaso asaluni kungotchulako ochepa, zomwe zimathandiza anthu akumudzi ambiri | Female | |
koma poyankhapo nduna ya za magetsi a Matola anati akudziwa bwino za vutoli ndipo posachedwa akoza vutoli kuti anthu apeze mwayi wa magetsi | koma poyankhapo nduna ya za magetsi a Matola anati akudziwa bwino za vutoli ndipo posachedwa akoza vutoli kuti anthu apeze mwayi wa magetsi | Female | |
Koma a Kanyama anati sakukhutirabe ndi zomwe ayankha anduna kuti apite ku wamkulu wa zoona za magetsi ku dera kwao zomwe yankholi lakhala likuyankhidwa kwa zaka ziwiri koma zithu sizikutheka | Koma a Kanyama anati sakukhutirabe ndi zomwe ayankha anduna kuti apite ku wamkulu wa zoona za magetsi ku dera kwao zomwe yankholi lakhala likuyankhidwa kwa zaka ziwiri koma zithu sizikutheka | Female | |
Koma iye anati monga phungu amene anthu amudera lawo anamutuma kukawaimilira kunyumba ya malamulo ayesetsa kuchita chilichonse kuti magetsi abwere | Koma iye anati monga phungu amene anthu amudera lawo anamutuma kukawaimilira kunyumba ya malamulo ayesetsa kuchita chilichonse kuti magetsi abwere | Female | |
Ndipo anapitiliza kunena kuti anafusa ndunayi kuti asithe transformer yomwe anaika mbuyomu ponena kuti inali yopanda mphamvu yomwe imakanika kukoka zithu zina | Ndipo anapitiliza kunena kuti anafusa ndunayi kuti asithe thilansifoma yomwe anaika mbuyomu ponena kuti inali yopanda mphamvu yomwe imakanika kukoka zithu zina | Female | |
Phungu wanyumba ya malamulo wa chigawo cha pakati m'boma la Chikwawa a Salim Bagus ati Boma likuyenera kuti lichite machawi pothandiza anthu ama boma a Chikwawa ndi ndi Nsanje omwe ankhudziwa ndi njala | Phungu wanyumba ya malamulo wa chigawo cha pakati m'boma la Chikwawa a Salimu Bagasi ati Boma likuyenera kuti lichite machawi pothandiza anthu ama boma a Chikwawa ndi ndi Nsanje omwe ankhudziwa ndi njala | Female | |
kamba ka ngozi za madzi osefukila zomwe zinankhudza mbomawa. Poyankhula ndi Angaliba online Salim Bagus anati pano ku Chikwawa kuli njala yambiri | kamba ka ngozi za madzi osefukila zomwe zinankhudza mbomawa. Poyankhula ndi Angaliba onilaini Salimu Bagasi anati pano ku Chikwawa kuli njala yambiri | Female | |
anthu akuvutika kwambiri boma likuyenera kuchitapo kathu msanga powabweretsera Chimanga chokwanila. Chikwawa ndi dera limodzi lomwe linankhudwa ndi madzi osefukila chaka chino | anthu akuvutika kwambiri boma likuyenera kuchitapo kathu msanga powabweretsera Chimanga chokwanila. Chikwawa ndi dera limodzi lomwe linankhudwa ndi madzi osefukila chaka chino | Female | |
Phungu wa nyumba ya Malamulo wa dera la Nsanje Lalanje komanso ndi wapampando wa komiti yoona za chuma mnyumba ya malamulo a Gladys Ganda | Phungu wa nyumba ya Malamulo wa dera la Nsanje Lalanje komanso ndi wapampando wa komiti yoona za chuma mnyumba ya malamulo a Giladesi Ganda | Female | |
wati Boma likuyenera kupeza njira zabwino zokwezera Chuma cha dziko lino chimene chapita pansi kwambiri pamene zithu zafika povuta | wati Boma likuyenera kupeza njira zabwino zokwezera Chuma cha dziko lino chimene chapita pansi kwambiri pamene zithu zafika povuta | Female | |
Ganda amayankhula izi pamene wasankhidwanso kukhala wapampando mu komiti yoona za chuma ya nyumba ya malamulo, Iye anati ayesetsa kugwira ntchito ndi boma | Ganda amayankhula izi pamene wasankhidwanso kukhala wapampando mu komiti yoona za chuma ya nyumba ya malamulo, Iye anati ayesetsa kugwira ntchito ndi boma | Female | |
komanso kuunikilapo za mmene angachitire kuti chuma cha dziko chiyambirenso kuyenda bwino kuti anthu amene akuwatumikila mmadera akwao athe kumasangalala podziwa kuti akuphika kwambiri | komanso kuunikilapo za mmene angachitire kuti chuma cha dziko chiyambirenso kuyenda bwino kuti anthu amene akuwatumikila mmadera akwao athe kumasangalala podziwa kuti akuphika kwambiri | Female | |
Ganda anapitiliza kuti iwo ngati komiti ayesetsaso kuyankhula ndi mabungwe amene amathandiza dziko lino kuti aganizilenso njira zina zofuna kukweza chuma | Ganda anapitiliza kuti iwo ngati komiti ayesetsaso kuyankhula ndi mabungwe amene amathandiza dziko lino kuti aganizilenso njira zina zofuna kukweza chuma | Female | |
ngakhale kuti mavuto ena ndi adziko lonse lapansi. Koma iye anati ngakhale mavuto azachuma avuta koma awonetsetsa kuti zitukuko zina za dziko zomwe zimadzera ku thumba la chitukuko mu nyumba ya malamulo | ngakhale kuti mavuto ena ndi adziko lonse lapansi. Koma iye anati ngakhale mavuto azachuma avuta koma awonetsetsa kuti zitukuko zina za dziko zomwe zimadzera ku thumba la chitukuko mu nyumba ya malamulo | Female | |
zipitilire chifukwa ndi njira yonkhayo yomwe anthu akumidzi amapezerapo phindu mu njira zambiri ndipo ndi khumbo lake kuti ndalama yomwe ili pano ikadaonjezeledwa potsatira kugwa mphamvu kwa ndalama ya kwacha | zipitilire chifukwa ndi njira yonkhayo yomwe anthu akumidzi amapezerapo phindu mu njira zambiri ndipo ndi khumbo lake kuti ndalama yomwe ili pano ikadaonjezeledwa potsatira kugwa mphamvu kwa ndalama ya kwacha | Female | |
Ndipo iye ananenaso kuti akadakakonda kuti boma lichilimike pofuna kuonetsetsa kuti komwe kumachoka ndalama ku bungwe lotolera ndalama za boma kudzera ku misonkho aikileko chidwi | Ndipo iye ananenaso kuti akadakakonda kuti boma lichilimike pofuna kuonetsetsa kuti komwe kumachoka ndalama ku bungwe lotolera ndalama za boma kudzera ku misonkho aikileko chidwi | Female | |
kuti ngati dziko tidzitha kutolera ndalama zambiri pofuna kukweza chuma cha dziko chifukwa kumeneko ndiye kumakoka ndalama zoyendetsera dziko | kuti ngati dziko tidzitha kutolera ndalama zambiri pofuna kukweza chuma cha dziko chifukwa kumeneko ndiye kumakoka ndalama zoyendetsera dziko | Female | |
Ganda anati iye ndi wodzipereka kugwilira ntchito a Malawi onse amene anatuma kukawaimilira ku nyumba ya malamulo | Ganda anati iye ndi wodzipereka kugwilira ntchito a Malawi onse amene anatuma kukawaimilira ku nyumba ya malamulo | Female | |
Pamene Boma lili pakalikiliki kumanga ndi kukozanso miseu ina ya mimzinda ndi ma tauni kudzera muunduna woona zomangamanga | Pamene Boma lili pakalikiliki kumanga ndi kukozanso miseu ina ya mimzinda ndi ma tauni kudzera muunduna woona zomangamanga | Female | |
zadziwika kuti ndalama zokwana 8.9 billion zomwe zimayenera kugwira ntchito yokozanso minseu ina ya mu mzinda wa Blantyre, kudzera ku Khonsolo ya Mzinda wa Blantyre | zadziwika kuti ndalama zokwana eiti pointi naili Biliyoni zomwe zimayenera kugwira ntchito yokozanso minseu ina ya mu mzinda wa Bulantaya, kudzera ku Khonsolo ya Mzinda wa Bulantaya | Female | |
sinagwire ntchito yake ndipo sizikudziwika komwe zinapita. Izi zadziwika pomwe nduna yoona zomangamanga a Jacob Hara imayankhapo mu nyumba ya malamulo nthawi yamafunso, phungu wa nyumba ya malamulo a Ishmael Mkumba | sinagwire ntchito yake ndipo sizikudziwika komwe zinapita. Izi zadziwika pomwe nduna yoona zomangamanga a Jacobo Hara imayankhapo mu nyumba ya malamulo nthawi yamafunso, phungu wa nyumba ya malamulo a Ishumaeli Mkumba | Female | |
a dera la Blantyre Malabada anafunsa pofuna kudziwa kuti ndalama zokwana 500 million yomwe zinaperekedwa mu 2020 zomangila nseu wa tala wa Matayala- Anglican Chinseu, kuti zinapita kuti poti ntchito sinayambe | a dera la bulantaya Malabada anafunsa pofuna kudziwa kuti ndalama zokwana faifi handede miliyono yomwe zinaperekedwa mu twente twente zomangila nseu wa tala wa Matayala- Angilikani Chinseu, kuti zinapita kuti poti ntchito sinayambe | Female | |
Koma nduna yoona zomangamangayi a Hala anati izi akafuse ku khosolo ya mzinda wa Blantyre chifukwa Boma linapereka kale ndalama yogwilira ntchitoyi | Koma nduna yoona zomangamangayi a Hala anati izi akafuse ku khosolo ya mzinda wa Bulantaya chifukwa Boma linapereka kale ndalama yogwilira ntchitoyi | Female | |
Ndipo Angaliba itayankhula ndi phungu wa dera la Blantyre Malabada ati iye ayesetsa kulondoloza za nkhaniyi chifukwa ndi chofuna cha anthu a derali kuti ankhale ndi nseu wamakono | Ndipo Angaliba itayankhula ndi phungu wa dera la Bulantaya Malabada ati iye ayesetsa kulondoloza za nkhaniyi chifukwa ndi chofuna cha anthu a derali kuti ankhale ndi nseu wamakono | Female | |
chifukwa anthu ena akuona ngati phunguyu ndiye anasokoneza ndalamazi komaso anthu a derali akuganizila zokayenda pa nseu kuti adziwe chilungamo cha nkhaniyi kuti ndalama zinayenda bwanji | chifukwa anthu ena akuona ngati phunguyu ndiye anasokoneza ndalamazi komaso anthu a derali akuganizila zokayenda pa nseu kuti adziwe chilungamo cha nkhaniyi kuti ndalama zinayenda bwanji | Female | |
Ishmaeli Mkumba ndiye phungu wa dera la Blantyre – Malabada. Msaiwale Kavina Phiri yemwe ndi mwini wake wa Champions Stadium bwalo la zamasewera la makono ku Mponera m'boma la Dowa | Ishumaeli Mkumba ndiye phungu wa dera la Bulantaya – Malabada. Msaiwale Kavina Phiri yemwe ndi mwini wake wa Tchampiyonzi sitediyamu bwalo la zamasewera la makono ku Mponera m'boma la Dowa | Female | |
wati akufunitsitsa kuti kuno kwathu ku Malawi kukhale mabwalo a zamasewero apamwamba ngati njira imodzi yotukulira masewera ampira | wati akufunitsitsa kuti kuno kwathu ku Malawi kukhale mabwalo a zamasewero apamwamba ngati njira imodzi yotukulira masewera ampira | Female | |
Kavina yemwe wamanga bwalo lomwe likutenga chikoka cha ma team ambiri kamba ka maonekedwe a pamwamba, lomwe anatsegulira kale pa masewera omwe analipo pakati pa team ya Kamuzu Barracks ndi team ya Mukuru Wanderers | Kavina yemwe wamanga bwalo lomwe likutenga chikoka cha ma timu ambiri kamba ka maonekedwe a pamwamba, lomwe anatsegulira kale pa masewera omwe analipo pakati pa timu ya Kamuzu Balakisi ndi timu ya Mukuru Wandilazi | Female | |
panali khwimbi la anthu ndipo mlendo wolemekezeka anali nduna ya achinyama ndi za masewero a Richard Chimwendo Banda | panali khwimbi la anthu ndipo mlendo wolemekezeka anali nduna ya achinyama ndi za masewero a Litchadi Chimwendo Banda | Female | |
Poyankhula pa mwambo wotsegulira bwaloli Kavina wati akufunitsitsa kuti bwaloli likhale ngati la Bingu ndipo pomatha chaka chino zithu zambiri zikhala zitasithapo, ndipo pano akumanga malo ovalira ochita masewero | Poyankhula pa mwambo wotsegulira bwaloli Kavina wati akufunitsitsa kuti bwaloli likhale ngati la Bingu ndipo pomatha chaka chino zithu zambiri zikhala zitasithapo, ndipo pano akumanga malo ovalira ochita masewero | Female | |
chifukwa nkhani ya malo ozathandizila, chifukwa nkhani ya malo ozithandizira inatha kale. Kavina anapitiliza kunena kuti kutsatira kutsekedwa kwa mabwalo a Civo ndi Silver | chifukwa nkhani ya malo ozathandizila, chifukwa nkhani ya malo ozithandizira inatha kale. Kavina anapitiliza kunena kuti kutsatira kutsekedwa kwa mabwalo a sivo ndi Siliva | Female | |
ma team a Kamuzu Barracks ndi Civil service United apepha kale zofuna kumagwilitsira bwaloli kuti adzisewerera ngati pakhomo | ma team a Kamuzu Balakisi ndi sivo sevisi yunaitedi apepha kale zofuna kumagwilitsira bwaloli kuti adzisewerera ngati pakhomo | Female | |
koma iye anati zonse zili mchimake akungodikila kuti mabungwe a FAM ndi SULOM akayendele ndi kuwavomeleza kuti angathe kuchititsa masewera a league kapena zikho zina | koma iye anati zonse zili mchimake akungodikila kuti mabungwe a FAMU ndi SULOMU akayendele ndi kuwavomeleza kuti angathe kuchititsa masewera a lIGI kapena zikho zina | Female | |
Kavina anati pompano bwalori likhala likuchititsa masewera ngakhale akunja kufuna kuti anthu adziona maluso osiyanasiyana | Kavina anati pompano bwalori likhala likuchititsa masewera ngakhale akunja kufuna kuti anthu adziona maluso osiyanasiyana | Female | |
Koma Kavina wauza anthu aku Mponera ndi madera wozungulira kuti anthu akuyenera kugwilana manja ndi kuchitira zithu limodzi kamba koti bwaloli lithandiza anthu ambiri amalonda osiyanasiyana ndi madera onse ozungulira | Koma Kavina wauza anthu aku Mponera ndi madera wozungulira kuti anthu akuyenera kugwilana manja ndi kuchitira zithu limodzi kamba koti bwaloli lithandiza anthu ambiri amalonda osiyanasiyana ndi madera onse ozungulira | Female | |
Iye anapereka Chitsazo kuti malonda monga a zakudya, malo ogona, ndi akabaza, kungotchulapo ochebacha, kungotchulapo wochepa chabe kuti akhala akupindula kwambiri | Iye anapereka Chitsazo kuti malonda monga a zakudya, malo ogona, ndi akabaza, kungotchulapo ochebacha, kungotchulapo wochepa chabe kuti akhala akupindula kwambiri | Female | |
iye anatiso anthu ena akhala akupeza mwayi wa ntchito zosiyanasiyana chifukwa cha kubwera kwa bwalori, ntchito monga za ulonda, zomangamanga komanso zokoza pamalowa | iye anatiso anthu ena akhala akupeza mwayi wa ntchito zosiyanasiyana chifukwa cha kubwera kwa bwalori, ntchito monga za ulonda, zomangamanga komanso zokoza pamalowa | Female | |
kungotchulapo zochepa chabe kuti anthu adelari akhala akupindula. Pamene dziko la Malawi likupitilizabe zonkozekera za African Union Region 5 youth games | kungotchulapo zochepa chabe kuti anthu adelari akhala akupindula. Pamene dziko la Malawi likupitilizabe zonkozekera za Afulikani uniyoni lijoni faifi yufi gemuzi | Female | |
wapampando wa bungwe lomwe likukonza Za masewera a Denis Mombera wati atolankhani ndiye mtima wazochitika zonsezi pofuna kuzindikilitsa anthu muzochitikazi | wapampando wa bungwe lomwe likukonza Za masewera a Denisi Mombera wati atolankhani ndiye mtima wazochitika zonsezi pofuna kuzindikilitsa anthu muzochitikazi | Female | |
Izi amayankhula pamene anakoza nkumano wa atolankhani mu mzinda wa Lilongwe pofuna kuwazindikilitsa za udindo wawo Komaso mmene angaperekere ma uthenga kwa anthu | Izi amayankhula pamene anakoza nkumano wa atolankhani mu mzinda wa Lilongwe pofuna kuwazindikilitsa za udindo wawo Komaso mmene angaperekere ma uthenga kwa anthu | Female | |
Poyankhulapo a Mombera anati a Malawi akuyenera kudziwa za masewera amenewa ndicholinga choti adzathe kumabwera kudzapanga sapoti dziko lawo pamene akutenga nawo mbari zosiyanasiyana pamasewerawa | Poyankhulapo a Mombera anati a Malawi akuyenera kudziwa za masewera amenewa ndicholinga choti adzathe kumabwera kudzapanga sapoti dziko lawo pamene akutenga nawo mbari zosiyanasiyana pamasewerawa | Female | |
monga ife amene tikulandira alendo. Ndipo wa mkulu mu unduna wa za achinyamata ndi masewero a Jameson Ndalama anati Malawi ngati dziko lipindula Kwambiri kumbali ya zithu zosiyanasiyana | monga ife amene tikulandira alendo. Ndipo wa mkulu mu unduna wa za achinyamata ndi masewero a Jamusoni Ndalama anati Malawi ngati dziko lipindula Kwambiri kumbali ya zithu zosiyanasiyana | Female | |
monga kukhala ndi mabwalo apamwamba womwe angamatibweretsere ndalama, ndi zina.Ndipo anapitiliza kunena kuti anthu amene akubwera kuno Kwathu ndiwosachepera 2500 | monga kukhala ndi mabwalo apamwamba womwe angamatibweretsere ndalama, ndi zina.Ndipo anapitiliza kunena kuti anthu amene akubwera kuno Kwathu ndiwosachepera thu sauzande faifi handede | Female | |
Masewera amenewa ndi achinyamata achisodzera ndipo akuyembekezeka kudzayamba mu mwezi wa December ndipo ife ngati dziko tapatsidwa kuti pofika mwezi wa October tikhale Kuti tamaliza zokozekera ku nkhani ya zomangamanga | Masewera amenewa ndi achinyamata achisodzera ndipo akuyembekezeka kudzayamba mu mwezi wa Disemba ndipo ife ngati dziko tapatsidwa kuti pofika mwezi wa Okotoba tikhale Kuti tamaliza zokozekera ku nkhani ya zomangamanga | Female | |
Maiko omwe akuyembekeza kufika ndi monga; Lesontho, Angola, Botswana, Eswatin, Mozambique, Namibia, Namibia. South Africa, Zambia, ndi Zimbabwe | Maiko omwe akuyembekeza kufika ndi monga; Lesontho, Angola, Botswana, Eswatini, Mozambiki, Namibiya, Namibiya. Saufi afilika, Zambia, ndi Zimbabwe | Female | |
Ndipo masewera omwe akuyembekezeka kudzachitika ndi monga; Football, netball, volleyball, basketball, Taekwando, Judo, Tenis kungotchulapo zochepa chabe | Ndipo masewera omwe akuyembekezeka kudzachitika ndi monga futubo, netibo, volebo, basiketibo, taikwando, judo, tenisi kungotchulapo zochepa chabe | Female | |
Unduna wa za umoyo wati uyambaso ntchito yopeleka katemera wa poliyo mu gawo lachitatu la kampeni yothana ndi kufala kwa mliliwu | Unduna wa za umoyo wati uyambaso ntchito yopeleka katemera wa poliyo mu gawo lachitatu la kampeni yothana ndi kufala kwa mliliwu | Female | |
Mu chikalata chomwe undunawu watulusa kudzera mu nthambi ya zaumoyo chomwe wasainila ndi mkulu wa zaumoyo m'bomali a Gift Kawalazila | Mu chikalata chomwe undunawu watulusa kudzera mu nthambi ya zaumoyo chomwe wasainila ndi mkulu wa zaumoyo m'bomali a Gifiti Kawalazila | Female | |
ati ana onse osapyola zaka zisanu ndiomwe akuyenera kulandira katemelayu posatengera kuti analandira kale | ati ana onse osapyola zaka zisanu ndiomwe akuyenera kulandira katemelayu posatengera kuti analandira kale | Female | |
Mkulu wa masapota a mighty mukuru wanderes mchigawo cha pakati a Rodrick Chitedze wati team yawo ndi yabwinobwino ndipo itha kuchita bwino kwambiri ponkhaponkha ngati anthu onse atagwirana manja ndi kuchepetsa mabodza pakati pawo | Mkulu wa masapota a maite mukuru wandilazi mchigawo cha pakati a lodiliki Chitedze wati timu yawo ndi yabwinobwino ndipo itha kuchita bwino kwambiri ponkhaponkha ngati anthu onse atagwirana manja ndi kuchepetsa mabodza pakati pawo | Female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.