audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Nayo Namitete Zitha FC ayipeza yolakwa kuti akuluakulu ake ena ankalankhula ndi osewera a Ngolowindo FC
Nayo Namitete Zitha efusi ayipeza yolakwa kuti akuluakulu ake ena ankalankhula ndi osewera a Ngolowindo efusi
Female
Pakadali pano, Central Region Football Association yatsimikiza kuti masewero a pakati pa ma timu a Kawinga FC ndi Namitete Zitha FC
Pakadali pano, sentilo lijoni futubo asosiyeshoni yatsimikiza kuti masewero a pakati pa ma timu a Kawinga efusi ndi Namitete Zitha efusi
Female
amene inawayimitsa pa 14 Januwale, nkhaniyi ya chinyengoyi itaphulika, aseweredwa la mulungu, pa 28 Januwale pa bwalo la Nankhaka ku Lilongwe
amene inawayimitsa pa fotini Januwale, nkhaniyi ya chinyengoyi itaphulika, aseweredwa la mulungu, pa twente eiti Januwale pa bwalo la Nankhaka ku Lilongwe
Female
Nzika zokhudzidwa pa chitukuko ku dera la Ntonda pansi pa INkosi Phambala m’boma la Ntcheu zadandaula ndikusowa kwa galimoto
Nzika zokhudzidwa pa chitukuko ku dera la Ntonda pansi pa INkosi Phambala m’boma la Ntcheu zadandaula ndikusowa kwa galimoto
Female
Nzika zokhudzidwa pa chitukuko ku dera la Ntonda pansi pa INkosi Phambala m’boma la Ntcheu zadandaula ndikusowa kwa galimoto
Nzika zokhudzidwa pa chitukuko ku dera la Ntonda pansi pa INkosi Phambala m’boma la Ntcheu zadandaula ndikusowa kwa galimoto
Female
yonyamula odwala pa chipatala chaching’ono cha Kapeni m’bomalo ponena kuti izi zikusokoneza ntchito za umoyo mderalo
yonyamula odwala pa chipatala chaching’ono cha Kapeni m’bomalo ponena kuti izi zikusokoneza ntchito za umoyo mderalo
Female
M’modzi wa nzikazi kudzera ku Liwu la Nzika a Zomba Banda wati chipatalachi chimathandiza anthu oposa 70,000
M’modzi wa nzikazi kudzera ku Liwu la Nzika a Zomba Banda wati chipatalachi chimathandiza anthu oposa sevente sauzande
Female
koma chikumadalira galimoto la mtunduwu lomwe limachokera ku chipatala chachikulu cha bomalo chomwe chili pa mtunda wa makilomita pafupipafupi 30
koma chikumadalira galimoto la mtunduwu lomwe limachokera ku chipatala chachikulu cha bomalo chomwe chili pa mtunda wa makilomita pafupipafupi fete
Female
Wachiwiri kwa wapampando wa khonsolo ya boma la Ntcheu, Khansala Stella Mpaso wati ndondomeko ili mkati kuti atumizeko galimoto lonyamula anthu odwala pachipatalachi
Wachiwiri kwa wapampando wa khonsolo ya boma la Ntcheu, Khansala Sitela Mpaso wati ndondomeko ili mkati kuti atumizeko galimoto lonyamula anthu odwala pachipatalachi
Female
Pakadali pano, m’modzi wa akuluakulu ku bungwe la World Vision Malawi kuchigawo chakum’mwera a Takondwa Mwale wati ndiosangalala kuti nzika zikutha kulondoloza adindo pankhani zachitukuko
Pakadali pano, m’modzi wa akuluakulu ku bungwe la waodi vizyoni Malawi kuchigawo chakum’mwera a Takondwa Mwale wati ndiosangalala kuti nzika zikutha kulondoloza adindo pankhani zachitukuko
Female
Lachisanu, nzikazi zinaitanitsa adindo m’bomalo kuti ayankhepo mafunso pamavuto omwe akukumana nawo kuderalo pa nkhani za umoyo komanso maphunziro ndi zina
Lachisanu, nzikazi zinaitanitsa adindo m’bomalo kuti ayankhepo mafunso pamavuto omwe akukumana nawo kuderalo pa nkhani za umoyo komanso maphunziro ndi zina
Female
Malo otsika mtengo ndi olipira pang'onopang'ono akupezekabe ku Citizen Real Estate Company. Muli ndi mwayi ogula plot panokha, kapena kudzera m'magulu a Bank Mkhonde
Malo otsika mtengo ndi olipira pang'onopang'ono akupezekabe ku sitizeni lilu esiteti kampane. Muli ndi mwayi ogula puloti panokha, kapena kudzera m'magulu a Banki Mkhonde
Female
ndi mzipereganyu zogulirana malo olipira pang'onopang'ono mwezi uliwonse kwa miyezi 12 chaka chonse cha 2024
ndi mzipereganyu zogulirana malo olipira pang'onopang'ono mwezi uliwonse kwa miyezi thwelofu chaka chonse cha twente twente folo
Female
Bwerani ku office kwathu pa Wakawaka kuti mudzaone mwaulere ndikusankha ma plot akumtima kwanu
Bwerani ku ofesi kwathu pa Wakawaka kuti mudzaone mwaulere ndikusankha ma puloti akumtima kwanu
Female
Khonsolo ya boma la Dedza lero yagawa matumba 640 a chimanga kwa anthu omwe akhudzika ndi njala dera la mfumu yayikulu Kamenyagwaza m'bomali
Khonsolo ya boma la Dedza lero yagawa matumba sikisi handiledi andi fote a chimanga kwa anthu omwe akhudzika ndi njala dera la mfumu yayikulu Kamenyagwaza m'bomali
Female
DC wa bomali la a Thomas Chigwenembe wauza Zodiak kuti ntchito yogawa chimangayi akwanitsa kufikira mabaanja 44,000 madera onse m'bomali
Disi wa bomali la a Thomasi Chigwenembe wauza Zodiyaki kuti ntchito yogawa chimangayi akwanitsa kufikira mabaanja fotefolo sauzande madera onse m'bomali
Female
Mfumu yayikulu Kamenyagwaza yathokoza boma kaamba ka thandizoli ndipo yapempha mabungwe kuti nawonso athandize kaamba koti anthu omwe akhudzika ndi njala ndi ambiri
Mfumu yayikulu Kamenyagwaza yathokoza boma kaamba ka thandizoli ndipo yapempha mabungwe kuti nawonso athandize kaamba koti anthu omwe akhudzika ndi njala ndi ambiri
Female
Phungu wa nyumba ya malamulo kumwera chakuvuma kwa boma la Kasungu, Khumbize Kandodo Chiponda walangiza achinyamata kuti atengerepo mwayi wa ngongole ya boma ya NEEF potukula miyoyo yao kudzera mmabizinesi
Phungu wa nyumba ya malamulo kumwera chakuvuma kwa boma la Kasungu, Khumbize Kandodo Chiponda walangiza achinyamata kuti atengerepo mwayi wa ngongole ya boma ya Nifi potukula miyoyo yao kudzera mmabizinesi
Female
Iwo alankhula izi potsatira zomwe achinyamata a gulu la la Chisomo 3, mdera la Mfumu Chambwe achitira umboni kuti kudzera ku phindu lomwe apeza
Iwo alankhula izi potsatira zomwe achinyamata a gulu la la Chisomo fili, mdera la Mfumu Chambwe achitira umboni kuti kudzera ku phindu lomwe apeza
Female
kuchokera ku ngongole ya Neef, akwanitsa kugula galimoto komanso njinga za moto Wapambando wa gululi, Rabson Kafunga
kuchokera ku ngongole ya Nifi, akwanitsa kugula galimoto komanso njinga za moto Wapambando wa gululi, Rabisoni Kafunga
Female
wati ngongoleyi chiongola dzanja chake mchochepa zomwe zathandiza kuti azitha kubweza mosavuta komanso kupeza phindu
wati ngongoleyi chiongola dzanja chake mchochepa zomwe zathandiza kuti azitha kubweza mosavuta komanso kupeza phindu
Female
A Chiponda omwenso ndi nduna ya za umoyo ati nthawi yomangogoma bao kapena kutaya nthawi ndi kuledzera idatha
A Chiponda omwenso ndi nduna ya za umoyo ati nthawi yomangogoma bao kapena kutaya nthawi ndi kuledzera idatha
Female
ndipo boma likupereka ngongoleyi kuti anthu athe kutukuka. Malinga ndi wapampando wa bungwe la NEEF, Jephter Mtema, boma la Kasungu lokha lapindula ndi ndalama zoposa K3.9 billion
ndipo boma likupereka ngongoleyi kuti anthu athe kutukuka. Malinga ndi wapampando wa bungwe la Nifi, Jefita Mtema, boma la Kasungu lokha lapindula ndi ndalama zoposa fili pointi naini biliyoni kwacha
Female
kuchokera mchaka cha 2021 mwa ndalama zokwana K87 billion zomwe NEEF yagawa dziko lonse
kuchokera mchaka cha twente twente wani mwa ndalama zokwana eite seveni biliyoni kwacha zomwe Nifi yagawa dziko lonse
Female
Ofesi yoona za nkhalango ku Dedza yati mitengo yokwana 1.6 miliyoni ndi yomwe akuyembekezera kudzala
Ofesi yoona za nkhalango ku Dedza yati mitengo yokwana wani pointi sikisi miliyoni ndi yomwe akuyembekezera kudzala
Female
chaka Chino m'bomali ndipo yapempha anthu m'bomali kuti aliyese adzale mitengo pa khomo pake
chaka Chino m'bomali ndipo yapempha anthu m'bomali kuti aliyese adzale mitengo pa khomo pake
Female
Ogwirizira Udindo wa mkulu wa zankhalango m'bomali a Carol Chidzungu awuza Zodiak kuti chaka chatha pa mitengo yokwana 1.6 miliyoni yomwe anadzala 70 peresenti ya mitengoyi inapulumuka
Ogwirizira Udindo wa mkulu wa zankhalango m'bomali a Karo Chidzungu awuza Zodiyaki kuti chaka chatha pa mitengo yokwana wani pointi sikisi miliyoni yomwe anadzala sevente peresenti ya mitengoyi inapulumuka
Female
Wapampando wa khonsolo ya Dedza a Themuka Nkhwewu wati ayika ndondomeko zoti mitengo yonse yomwe ikudzalidwa ipulumuke kuti nyengo yaku Dedza ibwerere mwa kale
Wapampando wa khonsolo ya Dedza a Themuka Nkhwewu wati ayika ndondomeko zoti mitengo yonse yomwe ikudzalidwa ipulumuke kuti nyengo yaku Dedza ibwerere mwa kale
Female
Gulu lina la amayi kwa mfumu yaikulu Kampingo Sibande kumpoto kwa boma la Mzimba lamanga chipatala chaching'ono komanso nyumba yokhalamo mlangizi
Gulu lina la amayi kwa mfumu yaikulu Kampingo Sibande kumpoto kwa boma la Mzimba lamanga chipatala chaching'ono komanso nyumba yokhalamo mlangizi
Female
ngati njila imodzi yowonesetsa kuti mwazina ana omwe sanathe zaka zisanu zakubadwa azitha kulandira katemera yense mosavuta
ngati njila imodzi yowonesetsa kuti mwazina ana omwe sanathe zaka zisanu zakubadwa azitha kulandira katemera yense mosavuta
Female
Yemwe akuyang'anila gululi a Mellifa Phiri wati ndithandizo la upangiri kuchokera kumgwilizano wamabungwe omwe amagwira ntchito zaumoyo la Malawi Health Equity Network
Yemwe akuyang'anila gululi a Mellifa Phiri wati ndithandizo la upangiri kuchokera kumgwilizano wamabungwe omwe amagwira ntchito zaumoyo la Malawi hefe ikwite netiweki
Female
iwo anafunsa unduna wazaumoyo kuti awapatse ogwila ntchito wazaumoyo yemwe awapatsa. Wachiwiri kwa nduna yaza umoyo a Harima Daud
iwo anafunsa unduna wazaumoyo kuti awapatse ogwila ntchito wazaumoyo yemwe awapatsa. Wachiwiri kwa nduna yaza umoyo a Harima Daudi
Female
wati ndipofunika kuti ntchitozi zifalikire mmadera ena kuti anthu ambiri athandizike mdzikolino
wati ndipofunika kuti ntchitozi zifalikire mmadera ena kuti anthu ambiri athandizike mdzikolino
Female
Bungwe la MHEN kudzera ku Boma likugwira ntchito yolimbikitsa komanso kupititsa patsogolo njila zolandilira katemera zomwe akuthandiza ndi a bungwe la GAVI
Bungwe la emuetchi ieni kudzera ku Boma likugwira ntchito yolimbikitsa komanso kupititsa patsogolo njila zolandilira katemera zomwe akuthandiza ndi a bungwe la GAVI
Female
Nduna yowona za Umoyo, Khumbize Kandodo Chiponda, yayamikira bungwe la Light House Trust kamba kowonjezera nthenda zina pamwamba HIV ndi AIDS
Nduna yowona za Umoyo, Khumbize Kandodo Chiponda, yayamikira bungwe la laiti hausi thilasiti kamba kowonjezera nthenda zina pamwamba etchiaivi ndi edzi
Female
imene bungweli yakhala ikuthandizira nkhondo yolimbana nayo chilikhazikitsireni. A Kandodo Chiponda ati izi zipeputsa zipatala za boma
imene bungweli yakhala ikuthandizira nkhondo yolimbana nayo chilikhazikitsireni. A Kandodo Chiponda ati izi zipeputsa zipatala za boma
Female
kamba koti zipatala za Light House zizithandizanso anthu odwala nthenda zina amene amadalira zipatala za boma zokha
kamba koti zipatala za laiti hausi zizithandizanso anthu odwala nthenda zina amene amadalira zipatala za boma zokha
Female
Ndunayi yalankhula izi ku Lilongwe pamene bungwe la Light House limalengeza kuti tsopano lidzithandizanso odwala nthenda zina monga cholera, kuyesetsa COVID-19
Ndunayi yalankhula izi ku Lilongwe pamene bungwe la laiti hausi limalengeza kuti tsopano lidzithandizanso odwala nthenda zina monga cholera, kuyesetsa kovidi naintini
Female
kuwunika komanso kupereka thandizo la khansa ya khomo la chibelekero, kuwunika komanso kupereka thandizo la nthenda ya TB, kuyeza nthenda ya mtima, malungo ndi nthenda zina
kuwunika komanso kupereka thandizo la khansa ya khomo la chibelekero, kuwunika komanso kupereka thandizo la nthenda ya Tibi, kuyeza nthenda ya mtima, malungo ndi nthenda zina
Female
Mkulu wa bungwe la Light House Trust, a Safari Mbewe, ati anthu ogwira ntchito ku zipatala za bungweli akonzeka kuwonjezera ukadaulo wawo kuti adzithandiza odwala mokwanira
Mkulu wa bungwe la laiti hausi thilasiti, a Safari Mbewe, ati anthu ogwira ntchito ku zipatala za bungweli akonzeka kuwonjezera ukadaulo wawo kuti adzithandiza odwala mokwanira
Female
Kupatulapo chipatala chachikulu chimene chili ku Kamuzu Central, bungwe la Light House Trust lirinso ndi nthambi zake mzipatala za Mzuzu, Bwaila, Queen Elizabeth ku Blantyre ndi Zomba
Kupatulapo chipatala chachikulu chimene chili ku Kamuzu sentilo, bungwe la Light House Trust lirinso ndi nthambi zake mzipatala za Mzuzu, Bwaila, kwini elizabefi ku Bulantaya ndi Zomba
Female
Bungweli limalandira thandizo la ndalama zokwana 13 million dollars za America pa chaka kuchokera ku bungwe la US Centers for Disease Control and Prevention
Bungweli limalandira thandizo la ndalama zokwana fetili miliyoni dolazi za Amerika pa chaka kuchokera ku bungwe la yuesi sentazi fo dizizi kontilo andi pulivenshoni
Female
Mkulu oimila boma pa milandu a Masauko Chamkakala, wathetsa mlandu omwe anthu ena atatu amayankha owaganizira kuti anatsekela njira mdipiti wa galimoto za mtsogoleri wa dziko lino
Mkulu oimila boma pa milandu a Masauko Chamkakala, wathetsa mlandu omwe anthu ena atatu amayankha owaganizira kuti anatsekela njira mdipiti wa galimoto za mtsogoleri wa dziko lino
Female
a Lazarus Chakwera pa HHI ku Blantyre lachisanu sabata yatha. Atatuwa, a Hector Ndawala a zaka 38, a Pearson Chimimba, azaka 48
a Lazalasi Chakwera pa etchi etchi ayi ku Bulantaya lachisanu sabata yatha. Atatuwa, a Hekita Ndawala a zaka fete eiti, a Piyasoni Chimimba, azaka fote eiti
Female
ndi mayi Lucy Namba, a zaka 25, ndiwo amayankha mlandu ndipo amayembekezeka kumva mawa lino chigamulo cha belo yomwe anapempha ku bwalo lamilandu
ndi mayi Luse Namba, a zaka twente faifi, ndiwo amayankha mlandu ndipo amayembekezeka kumva mawa lino chigamulo cha belo yomwe anapempha ku bwalo lamilandu
Female
Mwachidule, a Chamkakala anangoti, mlanduwu awuthetsa. Unduna woona za maiko ena wati wauza ofesi ya kazembe ya dziko lino ku India
Mwachidule, a Chamkakala anangoti, mlanduwu awuthetsa. Unduna woona za maiko ena wati wauza ofesi ya kazembe ya dziko lino ku Indiya
Female
kuti ifufuze malipoti oti mayi wina yemwe ndi mzika ya dziko lino amumanga ku Bangladesh poyiganizira kuti amazembetsa mankhwala ozunguza bongo a Cocain olemera makilo 8.3
kuti ifufuze malipoti oti mayi wina yemwe ndi mzika ya dziko lino amumanga ku Bangiladeshi poyiganizira kuti amazembetsa mankhwala ozunguza bongo a kokeni olemera makilo eiti pointi fili
Female
Nyumba zofalitsa nkhani mdzikolo zati achitetetezo amanga mayiyu, Nomthandazo Towera Soko wa zaka 35, lachinayi pa bwalo la ndege la Dhaka anthu ena atawatsina khutu
Nyumba zofalitsa nkhani mdzikolo zati achitetetezo amanga mayiyu, Nomthandazo Towera Soko wa zaka fete faifi, lachinayi pa bwalo la ndege la Dhaka anthu ena atawatsina khutu
Female
Dziko la Bangladesh lati mulingo wa mankhwala ozunguza bongowa ndi waukulu kwambiri mu mbiri ya dzikolo
Dziko la Bangiladeshi lati mulingo wa mankhwala ozunguza bongowa ndi waukulu kwambiri mu mbiri ya dzikolo
Female
Mneneri wa undunawu, John Kabaghe wati zomwe ofesi ya kazembeyi ipeze zithandiza kuti dziko lino lipange chiganizo pa nkhaniyi
Mneneri wa undunawu, Joni Kabange wati zomwe ofesi ya kazembeyi ipeze zithandiza kuti dziko lino lipange chiganizo pa nkhaniyi
Female
Bungwe lina la ntchito zachifundo la Henry for All Children Foundation lati lidzipeleka thandizo la maphunziro kwa ana achichepele okwana 30 omwe ndi amasiye
Bungwe lina la ntchito zachifundo la Henele fo otchudileni faundeshoni lati lidzipeleka thandizo la maphunziro kwa ana achichepele okwana fete omwe ndi amasiye
Female
m'mudzi mwa M'chambwe kwa Senior Chief Mphonde m'boma la Nkhotakota, kufikila anawo, atadzachita maphunziro a sekondale. M'modzi mwa akuluakulu a bungwelo, a Jonathan Mhango
m'mudzi mwa M'chambwe kwa Siniyo tchifi Mphonde m'boma la Nkhotakota, kufikila anawo, atadzachita maphunziro a sekondale. M'modzi mwa akuluakulu a bungwelo, a Jonathan Mhango
Female
wati izi zadza atazindikila kuti anawa akumachita maganyu m'minda pofuna kupeza ndalama zolipiilira zinthu zosiyanasiyana zokhudza maphunziro a m'sukulu za pulaimale
wati izi zadza atazindikila kuti anawa akumachita maganyu m'minda pofuna kupeza ndalama zolipiilira zinthu zosiyanasiyana zokhudza maphunziro a m'sukulu za pulaimale
Female
Lero bungweli lapeleka uniform kwa anawa. Senior Chief Mphonde ya m'bomalo ikuti izi ndi zosangalatsa potengela kuti ana ochuluka amasiye akuvutika pa maphunziro
Lero bungweli lapeleka unifomu kwa anawa. Siniyo tchifi Mphonde ya m'bomalo ikuti izi ndi zosangalatsa potengela kuti ana ochuluka amasiye akuvutika pa maphunziro
Female
ndipo yapempha anthu ndi magulu ena akufuna kwabwino kuti apelekenso thandizo lotele. Ziphaso zapepala zomwe Nthambi yoona zapansewu ya Directorate of Road Traffic and Safety Service.
ndipo yapempha anthu ndi magulu ena akufuna kwabwino kuti apelekenso thandizo lotele. Ziphaso zapepala zomwe Nthambi yoona zapansewu ya Dailekitoleti ofu lodi thilafiki andi sefete secisezi.
Female
ikupeleka m'malo mwa makhadi ati zikudzetsa udani pakati pa oyendetsa mini bus ndi apolisi
ikupeleka m'malo mwa makhadi ati zikudzetsa udani pakati pa oyendetsa minibasi ndi apolisi
Female
Oyendetsa minibusi mdela la Ndirande, mu mzinda wa Blantyre, a Evans Galasi, wauza pulezidenti Lazarus Chakwera kuti achitepo kanthu
Oyendetsa minibusi mdela la Ndirande, mu mzinda wa Bulantaya, a Evansi Galasi, wauza pulezidenti Lazalasi Chakwera kuti achitepo kanthu
Female
A Galasi ati m'malo oyimanso mini bus mu mzindawu salibwino, ndipo akadzionele okha
A Galasi ati m'malo oyimanso minibasi mu mzindawu salibwino, ndipo akadzionele okha
Female
Namtindi wamatelara, oyitanila minibasi, omanga tsitsi ndi kumeta, ochita geni ndi mavenda m'madela osiyana siyana mu mzinda wa Blantyre
Namtindi wamatelara, oyitanila minibasi, omanga tsitsi ndi kumeta, ochita geni ndi mavenda m'madela osiyana siyana mu mzinda wa Bulantaya
Female
akukumana ndi pulezidenti Lazarus Chakwera ku nyumba yachifumu ya Sanjika Palace
akukumana ndi pulezidenti Lazalasi Chakwera ku nyumba yachifumu ya Sanjika Palesi
Female
Akuluakulu pachipatala chamishoni cha Nkhoma ku Lilongwe ati mavuto akusowa kwa zipangizo zogwilira ntchito komanso kuchepa kwa ogwira ntchito
Akuluakulu pachipatala chamishoni cha Nkhoma ku Lilongwe ati mavuto akusowa kwa zipangizo zogwilira ntchito komanso kuchepa kwa ogwira ntchito
Female
akukhudza masomphenya awo ofuna kuthandiza anthu amadalira chipatalachi
akukhudza masomphenya awo ofuna kuthandiza anthu amadalira chipatalachi
Female
Mmodzi mwa akuluakulu oyendetsa ntchito zachipatalachi a Agnes Nyanda ndiwo anena izi lero
Mmodzi mwa akuluakulu oyendetsa ntchito zachipatalachi a Aginesi Nyanda ndiwo anena izi lero
Female
pomwe phungu wa dera lakumpoto m'boma la Dedza a Saviel Kafwafwa anakapereka thandizo la zinthu zosiyanasiyana zothandizira anthu odwala za ndalama zokwana K8 million
pomwe phungu wa dera lakumpoto m'boma la Dedza a Saviyelo Kafwafwa anakapereka thandizo la zinthu zosiyanasiyana zothandizira anthu odwala za ndalama zokwana eiti miliyoni kwacha
Female
Kupatula kupempha nthandizo kuchokera kwa akufuna kwabwino, a Nyanda apemphaso kuti ndalama zomwe boma limapereka kudzera pa mgwirizano oti chipatalachi chizithandiza anthu ammadera ena mwa ulele
Kupatula kupempha nthandizo kuchokera kwa akufuna kwabwino, a Nyanda apemphaso kuti ndalama zomwe boma limapereka kudzera pa mgwirizano oti chipatalachi chizithandiza anthu ammadera ena mwa ulele
Female
zikwele chifukwa chipatalachi chikuthandiza anthu ambiri kuchokera mmaboma ena. Ndipo polankhula atapereka thandizoli a Kafwafwa ati aganiza zothandiza chipatalachi
zikwele chifukwa chipatalachi chikuthandiza anthu ambiri kuchokera mmaboma ena. Ndipo polankhula atapereka thandizoli a Kafwafwa ati aganiza zothandiza chipatalachi
Female
pofuna kuchepetsako ena mwa mavuto ankhaninkhani omwe chikukumama nawo, kuti chipitilize kuthandiza odwala ochekera mmadera ena kuphatikizapo akudera lake
pofuna kuchepetsako ena mwa mavuto ankhaninkhani omwe chikukumama nawo, kuti chipitilize kuthandiza odwala ochekera mmadera ena kuphatikizapo akudera lake
Female
Ndipo a Kafwafwa alonjeza kuti atengera nkhani yokhudza kuonjezera thandizo mumgwirizano wa boma ndichipatalachi aphungu akakumana ku nyumba yamalamulo
Ndipo a Kafwafwa alonjeza kuti atengera nkhani yokhudza kuonjezera thandizo mumgwirizano wa boma ndichipatalachi aphungu akakumana ku nyumba yamalamulo
Female
Wina mwa katunduyu ndiwothandizira odwala malungo ndi chipinda chochilira amayi
Wina mwa katunduyu ndiwothandizira odwala malungo ndi chipinda chochilira amayi
Female
Atsogoleri azipembedzo zosiyanasiyana m’chigawo chakum’mwera awuza pulezidenti Lazarus Chakwera kuti asasiyile panjira ntchito yotsogolera dziko lino kuti akwanilitse masomphenya ake pachitukuko
Atsogoleri azipembedzo zosiyanasiyana m’chigawo chakum’mwera awuza pulezidenti Lazalasi Chakwera kuti asasiyile panjira ntchito yotsogolera dziko lino kuti akwanilitse masomphenya ake pachitukuko
Female
Yemwe anatsogolera atsogoleriwa Apostle Samuel Vikhumbo ndiwo anena izi atakumana ndi a Chakwera kunyumba yachifumu ya Sanjika ku Blantyre lero
Yemwe anatsogolera atsogoleriwa Aposito Samuyele Vikhumbo ndiwo anena izi atakumana ndi a Chakwera kunyumba yachifumu ya Sanjika ku Bulantaya lero
Female
Mlangizi wa a Chakwera pa nkhani zachipembedzo mbusa Brian Kamwendo, wati abusawa adzipelekanso kupemphelera utsogoleri wa a Chakwera
Mlangizi wa a Chakwera pa nkhani zachipembedzo mbusa Bulayani Kamwendo, wati abusawa adzipelekanso kupemphelera utsogoleri wa a Chakwera
Female
Anthu okhala dera la Kasinje mdera la INkosi Ganya m’boma la Ntcheu pansi pa Liwu la Nzika ayitanitsa adindo m’bomalo pamavuto omwe akukumana nawo kuderaro
Anthu okhala dera la Kasinje mdera la INkosi Ganya m’boma la Ntcheu pansi pa Liwu la Nzika ayitanitsa adindo m’bomalo pamavuto omwe akukumana nawo kuderaro
Female
Iwo akufuna mayankho ku mavuto aza maphunziro, umoyo, nkhani zoteteza ana komanso madzi ndi ukhondo
Iwo akufuna mayankho ku mavuto aza maphunziro, umoyo, nkhani zoteteza ana komanso madzi ndi ukhondo
Female
Wachiwiri kwa nduna ya zamaphunziro a Nancy Chaola Mdooko, DC wabomalo a George Ngaiyaye komanso mkulu wa zaumoyo m’boma la Ntcheu Dr. Emily Jenya
Wachiwiri kwa nduna ya zamaphunziro a Nanse Chaola Mdooko, Disi wabomalo a Joji Ngaiyaye komanso mkulu wa zaumoyo m’boma la Ntcheu Dokota. Emile Jenya
Female
ndi ena mwa adindo omwe afika pa msonkhanowu kuti ayankhe mafunso ndi mavutowa. Anthuwa ayitanitsa adindowa ndithandizo la bungwe la World Vision Malawi
ndi ena mwa adindo omwe afika pa msonkhanowu kuti ayankhe mafunso ndi mavutowa. Anthuwa ayitanitsa adindowa ndithandizo la bungwe la waodi vizyoni Malawi
Female
Apolisi amanga mwana wa wapolisi mzawo, Chifuniro Keith Manjolo, pomuganizira kuti amabera anthu atawanamiza kuti awapezera ntchito ku polisiko
Apolisi amanga mwana wa wapolisi mzawo, Chifuniro Kefi Manjolo, pomuganizira kuti amabera anthu atawanamiza kuti awapezera ntchito ku polisiko
Female
Woganizilidwayu, Manjolo akuti watchula dzina la wapolisi wa udindo wake ku Area 30, Assistant Commissioner of Police Joel Makiyi kuti ndiye amagwira naye ntchitoyi
Woganizilidwayu, Manjolo akuti watchula dzina la wapolisi wa udindo wake ku Area fete, Asisitanti Komishona ofu Polisi Jowelo Makiyi kuti ndiye amagwira naye ntchitoyi
Female
Manjolo, yemwe amayi ake amagwira ntchito kulikulu la polisi chigawo chapakati m'dera la chaku m'mawa m'boma la Kasungu
Manjolo, yemwe amayi ake amagwira ntchito kulikulu la polisi chigawo chapakati m'dera la chaku m'mawa m'boma la Kasungu
Female
poyamba anafusidwa ndi wapolisi wina kuti akafuse mayi ake kuti amuthandize kupezera ntchito mchimwene wake
poyamba anafusidwa ndi wapolisi wina kuti akafuse mayi ake kuti amuthandize kupezera ntchito mchimwene wake
Female
Pachiyambi, mwana wa apolisiyo anakana ponena kuti, mayi ake alibe mphamvu yopezera munthu ntchito
Pachiyambi, mwana wa apolisiyo anakana ponena kuti, mayi ake alibe mphamvu yopezera munthu ntchito
Female
Koma, patatha masiku akuti adamuyimbira wapolisiyo kumudziwitsa kuti wapeza njira yomuthandizira. Atatero, Manjolo anauza wapolisiyo kuti apereke 150 000
Koma, patatha masiku akuti adamuyimbira wapolisiyo kumudziwitsa kuti wapeza njira yomuthandizira. Atatero, Manjolo anauza wapolisiyo kuti apereke wani handiledi andi fifite sauzande
Female
Patapita masiku, anauzanso wapolisi ofuna thandizoyo, kuti malo a anthu ena asanu apezeka pa mtengo wa 180 000 kwacha
Patapita masiku, anauzanso wapolisi ofuna thandizoyo, kuti malo a anthu ena asanu apezeka pa mtengo wa wani handiledi andi eitesauzande kwacha
Female
Anthuwo anapereka ndalamazo, koma sipadathe masiku ambiri ndipo anazindikira kuti kalata zomwe anapatsidwa zinali zachinyengo, zomwe zachititsa kuti apolisi amange Manjolo
Anthuwo anapereka ndalamazo, koma sipadathe masiku ambiri ndipo anazindikira kuti kalata zomwe anapatsidwa zinali zachinyengo, zomwe zachititsa kuti apolisi amange Manjolo
Female
Gulu la alimi a Bomfa mdera la mfumu Mphomwa ku Kasungu likusimba lokoma litalandira thandizo la ndalama zoposa K84 miliyoni zotukulira ntchito zake
Gulu la alimi a Bomfa mdera la mfumu Mphomwa ku Kasungu likusimba lokoma litalandira thandizo la ndalama zoposa eite folo miliyoni kwacha zotukulira ntchito zake
Female
Thandizoli ndi mbali imodzi ya ndalama za mndondomeko ya Trade yomwe boma la Malawi ndi mabungwe a IFAD ndi Opec-fund akuthandiza magulu alimi kuti azitenga ulimi ngati businesi
Thandizoli ndi mbali imodzi ya ndalama za mndondomeko ya Thiledirade yomwe boma la Malawi ndi mabungwe a ifadi ndi Opeki-fandi akuthandiza magulu alimi kuti azitenga ulimi ngati businesi
Female
Zaina Kapachika wati ndalamazi zithandiza kuti gululi ligule makina amakono opangira mafuta oti lizitha kugulitsa ngakhale kunja kwa dziko lino
Zaina Kapachika wati ndalamazi zithandiza kuti gululi ligule makina amakono opangira mafuta oti lizitha kugulitsa ngakhale kunja kwa dziko lino
Female
Wapampando wa khonsolo ya Kasungu a Mwambiraso Mbedza ati mpamba wa bizinesi ndi chomwe alimi amasowa kuti azionjezera phindu pa ulimi
Wapampando wa khonsolo ya Kasungu a Mwambiraso Mbedza ati mpamba wa bizinesi ndi chomwe alimi amasowa kuti azionjezera phindu pa ulimi
Female
mwa akuluakulu a pulogram ya Trade a Linda Munthali ati ndalama zankhaninkhani zomwe magulu alimi apindule nazo m'maboma 11 mdziko muno
mwa akuluakulu a pulogram ya Thiledi a Linda Munthali ati ndalama zankhaninkhani zomwe magulu alimi apindule nazo m'maboma leveni mdziko muno
Female
Apolisi ku Lilongwe amanga wapolisi mzawo pomuganizira kuti anaba njinga zamoto ziwiri za apolisi amzake omwe amagwira nawo ntchito ku C Division
Apolisi ku Lilongwe amanga wapolisi mzawo pomuganizira kuti anaba njinga zamoto ziwiri za apolisi amzake omwe amagwira nawo ntchito ku si divizyoni
Female
Ofalitsa nkhani za apolisi ku Lilongwe a Hastings Chigalu wati oganizilidwayu Nokesi Kashitiyano
Ofalitsa nkhani za apolisi ku Lilongwe a Hesiting’izi Chigalu wati oganizilidwayu Nokesi Kashitiyano
Female
anaba njinga ina mmwezi wa December chaka chatha pomwe mwini wanjingayu analo kokagwira ntchito ku Area 10 munzinda wa Lilongwe
anaba njinga ina mmwezi wa Disemba chaka chatha pomwe mwini wanjingayu analo kokagwira ntchito ku eliya teni munzinda wa Lilongwe
Female
A Chigalu ati alimkati momupanikiza ndimafunso, wapolisi wina wamang’alaso kuti mkuluyu anabaso njinga yake mnjira ngati yomweyi
A Chigalu ati alimkati momupanikiza ndimafunso, wapolisi wina wamang’alaso kuti mkuluyu anabaso njinga yake mnjira ngati yomweyi
Female
A Nokesi Kashitiyano a zaka 31, amachokera mmudzi mwa Mgona mdera la T/A Tengani ku Nsanje
A Nokesi Kashitiyano a zaka fetewani, amachokera mmudzi mwa Mgona mdera la tie Tengani ku Nsanje
Female
Bungwe la Netball Association of Malawi ( NAM) lasankha otchinga kumbuyo wa kale wa timu ya Queens, Joana Kachilika, kukhala mphunzitsi watsopano wa timuyi
Bungwe la netibo asosiyeshoni ofu Malawi ( NAMU) lasankha otchinga kumbuyo wa kale wa timu ya kwinzi, Joana Kachilika, kukhala mphunzitsi watsopano wa timuyi
Female
AKachilika, amene anasiya kusewera mchaka cha 2021, ndipo pakadali pano akuphunzitsa timu ya Imosys NC, walowa mmalo mwa Peace Chawinga
AKachilika, amene anasiya kusewera mchaka cha twente leveni, ndipo pakadali pano akuphunzitsa timu ya imose enisi, walowa mmalo mwa Pisi Chawinga
Female
Osewera enanso a kale a timu ya Malawi Queens, Eleanor Mapulanga ndi Beatrice Mpinganjira, awasankha kukhala othandizira Kachilika
Osewera enanso a kale a timu ya Malawi kwinzi, Elena Mapulanga ndi Bitilisi Mpinganjira, awasankha kukhala othandizira Kachilika
Female
Kalata ya bungwe la NAM yatinso Christina Mkwanda amusankha kukhala mphunzitsi wa timu ya chisodzera, ya osewera osapyola zaka 21 ndipo omuthandizira ake ndi Cecilia Bondwe ndi Vincent Shombe
Kalata ya bungwe la NAMU yatinso Khilisitina Mkwanda amusankha kukhala mphunzitsi wa timu ya chisodzera, ya osewera osapyola zaka twente wani ndipo omuthandizira ake ndi sisiliya Bondwe ndi Vinisenti Shombe
Female
Rose Chinyama amusankha kukhala mphunzitsi wa timu inanso ya chisodzera, koma osewera ake osapyola zaka 20 ndipo omuthandizira ake ndi Tereza Chipolopolo komanso Elnes Kachama
Rozi Chinyama amusankha kukhala mphunzitsi wa timu inanso ya chisodzera, koma osewera ake osapyola zaka twente ndipo omuthandizira ake ndi Tereza Chipolopolo komanso Elnesi Kachama
Female
Pakadali pano, timu ya Queens ili pa number 6 pa mndandanda wa ma timu a dziko lonse
Pakadali pano, timu ya kwinzi ili pa namba sikisi pa mndandanda wa ma timu a dziko lonse
Female