audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Mkuluyi adzapita limodzi ndi Pondamali Tembo amene ndi othandizira wa mmbali komanso referee opuma, Duncan Lengani amene amusankha m'gulu la alangizi a oyimbira
Mkuluyi adzapita limodzi ndi Pondamali Tembo amene ndi othandizira wa mmbali komanso lifali opuma, Dankeni Lengani amene amusankha m'gulu la alangizi a oyimbira
Female
President Lazarus Chakwera wati anaona chofunikira kuti apite ndi mtsogoleri wa dziko la Zimbabwe, Emmerson Mnangagwa ku Comforzi Macadamia
President Lazalasi Chakwera wati anaona chofunikira kuti apite ndi mtsogoleri wa dziko la Zimbabwe, Emesoni Mnangagwa ku komfozi Makademiya
Female
ndi Tea Plantation komanso fakitale zake ku Thyolo, kuti amalonda a m'dziko la Zimbabwe adzaguleko
ndi Tiyi pulanteshoni komanso fakitale zake ku Thyolo, kuti amalonda a m'dziko la Zimbabwe adzaguleko
Female
President Chakwera wati mtedza wa makedemiya ndi Tea ndi zina mwa mbewu zodalilika popeza ndalama zakunja pambali pa fodya
Pulezidenti Chakwera wati mtedza wa makedemiya ndi Tiyi ndi zina mwa mbewu zodalilika popeza ndalama zakunja pambali pa fodya
Female
M'mawu ake president Mnangagwa yemwe akuyembekezeka kubwerera lero wayamikira Tea wa dziko lino kuti ndiwapamwamba
M'mawu ake pulezidenti Mnangagwa yemwe akuyembekezeka kubwerera lero wayamikira Tiyi wa dziko lino kuti ndiwapamwamba
Female
Bungwe la ochita malonda a chi Malawi la Black Indegionous Business Network la dandaula ndi kusowa chidwi kwa anthu omwe anakhudzika ndi namondwe wa Freddy choyamba ntchito za malonda osiyanasiyana
Bungwe la ochita malonda a chi Malawi la Bulaki indijinasi bizinesi netiweki la dandaula ndi kusowa chidwi kwa anthu omwe anakhudzika ndi namondwe wa Fulede choyamba ntchito za malonda osiyanasiyana
Female
Mkulu wa bungweli, Ketie Kamwangala wanena izi pomwe gululi limakapereka thandizo losiyanasiyana monga sopo, mafuta ophikira, shuga mwa zina kwa anthu opitilira makumi asanu ndi atatu
Mkulu wa bungweli, Keti Kamwangala wanena izi pomwe gululi limakapereka thandizo losiyanasiyana monga sopo, mafuta ophikira, shuga mwa zina kwa anthu opitilira makumi asanu ndi atatu
Female
a m'madera a gulupu Nsomera ndi Mpama ku Mbulumbudzi m'boma la Chiradzulu. Nthawi zina kuyamba bizinezi sikuthanthauza kukhala ndi ndalama koma chidwi chabe chofuna kuyamba bizineziyo
a m'madera a gulupu Nsomera ndi Mpama ku Mbulumbudzi m'boma la Chiradzulu. Nthawi zina kuyamba bizinezi sikuthanthauza kukhala ndi ndalama koma chidwi chabe chofuna kuyamba bizineziyo
Female
Izi zikutanthauza kuti ndi kandalama kochepa komwe timapeza,titha kuyamba bizinezi. Gululi laperekanso ndalama yokwanira K200, 000 kwa magulu awiriwa kuti ayambire geni
Izi zikutanthauza kuti ndi kandalama kochepa komwe timapeza,titha kuyamba bizinezi. Gululi laperekanso ndalama yokwanira thu handiledi sauzande kwacha kwa magulu awiriwa kuti ayambire geni
Female
Pambali pothokoza bungweli, a Maureen Kandulo ochokera kwa gulupu Mpama ati ngakhale anthuwa abweleranso m'ma kwawo
Pambali pothokoza bungweli, a Molini Kandulo ochokera kwa gulupu Mpama ati ngakhale anthuwa abweleranso m'ma kwawo
Female
akukumanabe ndi mavuto osiyanasiyana maka chakudya kamba koti ambiri mwa iwo akusungidwa ndi a chibale
akukumanabe ndi mavuto osiyanasiyana maka chakudya kamba koti ambiri mwa iwo akusungidwa ndi a chibale
Female
M’neneri David Mbewe wa mpingo wa Living Word Evangelistic Church sakubwera poyera ndikufotoka za tsogolo la chidwi chake
M’neneri Devidi Mbewe wa mpingo wa Living’i Waodi Evangelisitiki Tchetchi sakubwera poyera ndikufotoka za tsogolo la chidwi chake
Female
chofuna kudzapikisana nawo pa mpando wamtsogoleri wa dziko.lino pachisankho cha m'chaka cha 2025
chofuna kudzapikisana nawo pa mpando wamtsogoleri wa dziko.lino pachisankho cha m'chaka cha twente twente faifi
Female
Izi zikudza kutsatira a Mbewe atalengeza kuti atula pansi utsogoleri wa ma bungwe awiri omwe iwo anayambitsa a 'Freedom of Worship and Economics Liberation Movement komanso Prophetic Ministries Association of Malawi
Izi zikudza kutsatira a Mbewe atalengeza kuti atula pansi utsogoleri wa ma bungwe awiri omwe iwo anayambitsa a fulidomu ofu woshipi andi ikonomikisi libeleshoni muvumenti komanso Pulofetiki minisitilezi asosiyeshoni ofu Malawi
Female
Poyankhura ndi Zodiak mneneliyu yemwe anthu omutsatira kudzera ku bungwe lake la FOWEM akhala akumupempha kuti adzapikisane nawo pa utsogoleri wa dziko linowu
Poyankhura ndi Zodiyaki mneneliyu yemwe anthu omutsatira kudzera ku bungwe lake la FOWEMU akhala akumupempha kuti adzapikisane nawo pa utsogoleri wa dziko linowu
Female
wati watula pansi ma udindowa atachitako kumbali yake ndipo pakadali pano akufuna ayike chidwi chake ku ntchito za mpingo
wati watula pansi ma udindowa atachitako kumbali yake ndipo pakadali pano akufuna ayike chidwi chake ku ntchito za mpingo
Female
Mbuyomu mneneriyu anatsindika za chidwi chake chofuna kukonza ena mwa mavuto omwe anthu mdziko muno akukumana nawo
Mbuyomu mneneriyu anatsindika za chidwi chake chofuna kukonza ena mwa mavuto omwe anthu mdziko muno akukumana nawo
Female
Iye anadabwitsa anthu atawonetsa chidwi chofuna kupikisana nawo pa utsogoleri wa chipani chotsutsa cha DPP komanso kulengeza kuti walowa muchipani cha DPP
Iye anadabwitsa anthu atawonetsa chidwi chofuna kupikisana nawo pa utsogoleri wa chipani chotsutsa cha Dipipi komanso kulengeza kuti walowa muchipani cha Dipipi
Female
Pakadali pano katswiri yemwe amayankhurapo pa zochitika mdziko a Victor Chipofya wati pamafunika kuti mneneriyu
Pakadali pano katswiri yemwe amayankhurapo pa zochitika mdziko a Vikita Chipofya wati pamafunika kuti mneneriyu
Female
abwere poyera pazaganizoli ngati njira imodzi yofuna kuchotsa chikaiko pakati pa omutsatira ake
abwere poyera pazaganizoli ngati njira imodzi yofuna kuchotsa chikaiko pakati pa omutsatira ake
Female
Hassan Kajoke wabwenza K3.9 million ku timu ya Silver Strikers komanso walipira chindapusa cha 200,000 Kwacha ku bungwe la FAM
Hasani Kajoke wabwenza fili pointi naini miliyoni kwacha ku timu ya Siuva sitilaikazi komanso walipira chindapusa cha thu handiledi sauzande Kwacha ku bungwe la FAMU
Female
kaamba konyazitsa mbiri ya mpira wa miyendo posayina migwirizano iwiri ndi ma timu a Silver komanso Bullets
kaamba konyazitsa mbiri ya mpira wa miyendo posayina migwirizano iwiri ndi ma timu a Siuva komanso Buletsi
Female
Komiti ya bungweli, yoona za osewera Players Status Committee inalamula Kajoke kuti abwenze K3 million
Komiti ya bungweli, yoona za osewera puleyazi sitetasi komiti inalamula Kajoke kuti abwenze fili miliyoni kwacha
Female
imene analandira ku timu ya Silver ngati signing-on fee komanso 900,000 Kwacha ngati malipiro a miyezi iwiri January ndi February
imene analandira ku timu ya Siuva ngati saining’I oni fii komanso naini handiledi sauzande kwacha Kwacha ngati malipiro a miyezi iwiri Januwale ndi Febuluwale
Female
Dzulo linali tsiku lotsiriza la masiku asanu amene komitiyi inalamula Kajoke kubwenza ndalamazi ndipo mmodzi mwa ma membala a board
Dzulo linali tsiku lotsiriza la masiku asanu amene komitiyi inalamula Kajoke kubwenza ndalamazi ndipo mmodzi mwa ma membala a bodi
Female
ya timu ya Silver, a Crispin Gwalawala Siwande, watsimikiza kuti ndalamazi azipereka
ya timu ya Siuva, a khilisipini Gwalawala Siwande, watsimikiza kuti ndalamazi azipereka
Female
Izi zikutanthauza kuti Kajoke tsopano ndi mfulu ndipo ali pa mndandanda wa osewera amene mphunzitsi wa Bullets
Izi zikutanthauza kuti Kajoke tsopano ndi mfulu ndipo ali pa mndandanda wa osewera amene mphunzitsi wa Buletsi
Female
Kalisto Pasuwa, akuyembekezeka kukhala nawo pa ulendo wa ku Karonga kumene timuyi ikukasewera ndi Chitipa United mu TNM Super League ku mathero a sabata ino
Kalisto Pasuwa, akuyembekezeka kukhala nawo pa ulendo wa ku Karonga kumene timuyi ikukasewera ndi Chitipa yunaitedi mu tieniemu supa ligi ku mathero a sabata ino
Female
M'neneri wa polisi mboma la Mulanje Sergeant Innocent Moses wati, apolisi akuganizira kuti khansala wa dera la Muloza ku Mulanje Limbuli
M'neneri wa polisi mboma la Mulanje sajenti inosenti mozesi wati, apolisi akuganizira kuti khansala wa dera la Muloza ku Mulanje Limbuli
Female
a Gift Lottie Chitekwe, anazembetsa, kugwililira mpaka kupereka mimba kwa mtsikana wa zaka 16
a Gifiti loti Chitekwe, anazembetsa, kugwililira mpaka kupereka mimba kwa mtsikana wa zaka sikisitini
Female
A Moses atsimkizira Zodiak Online kuti khansalayu akumusunga pa polisi ya Mulanje
A Mozesi atsimkizira Zodiyaki Onilaini kuti khansalayu akumusunga pa polisi ya Mulanje
Female
M'neneri wa polisi-yu wati khansala Chitekwe aonekera mbwalo la milandu posachedwapa komwe akayankhe milandu iwiri yomwe ndi kugwilira mtsikana wachichepere ndi muzembetsa ndi kusunga mwana
M'neneri wa polisi-yu wati khansala Chitekwe aonekera mbwalo la milandu posachedwapa komwe akayankhe milandu iwiri yomwe ndi kugwilira mtsikana wachichepere ndi muzembetsa ndi kusunga mwana
Female
Ophunzira 20 ku Mangochi salemba nawo mayeso a JCE, kaamba koti aphunzitsi awo anawadyela ndalama zomwe amayenela kulipila mayesowa omwe ayamba lelo, lachiwiri
Ophunzira twente ku Mangochi salemba nawo mayeso a jeyi si i, kaamba koti aphunzitsi awo anawadyela ndalama zomwe amayenela kulipila mayesowa omwe ayamba lelo, lachiwiri
Female
Kutsatira izi, nduna yoona za Maphunziro a Madalitso Kambauwa Wirima yati ndi kofunika kuti makolo komanso ophunzira azindikire ndi kugwilitsa ntchito njira zamakono
Kutsatira izi, nduna yoona za Maphunziro a Madalitso Kambauwa Wirima yati ndi kofunika kuti makolo komanso ophunzira azindikire ndi kugwilitsa ntchito njira zamakono
Female
zomwe zinakhazikitsidwa polewa m'chitidwewu. M'mayeso ochoka ku pulayimale PSLCE omwe apitawa, ophunzira 120
zomwe zinakhazikitsidwa polewa m'chitidwewu. M'mayeso ochoka ku pulayimale piesi elisiii omwe apitawa, ophunzira wani handiledi andi twente
Female
analephela kulemba nawo mayesowa chifukwa chakuti aphunzitsi awo anawadyela ndalama zolipira mayeso
analephela kulemba nawo mayesowa chifukwa chakuti aphunzitsi awo anawadyela ndalama zolipira mayeso
Female
Akatswiri pa nkhani za chuma ndi ufulu wa anthu adzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kaamba kolephera kukwaniritsa lonjezo lawo pa nkhani ya maulendo akunja
Akatswiri pa nkhani za chuma ndi ufulu wa anthu adzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazalasi Chakwera kaamba kolephera kukwaniritsa lonjezo lawo pa nkhani ya maulendo akunja
Female
Mu November chaka chatha, mtsogoleri wa dziko linoyu analongosola ndondomeko zochepetsera kuonongeka kwa ndalama malingana ndi kuchepa mphamvu kwa ndalama ya kwacha ndi 44 peresenti
Mu Novemba chaka chatha, mtsogoleri wa dziko linoyu analongosola ndondomeko zochepetsera kuonongeka kwa ndalama malingana ndi kuchepa mphamvu kwa ndalama ya kwacha ndi fotefolo peresenti
Female
Mwazina a Chakwera adalengeza kuti ayimitsa maulendo awo akunja mpaka March, ngati njira yopulumutsira ndalama
Mwazina a Chakwera adalengeza kuti ayimitsa maulendo awo akunja mpaka Malichi, ngati njira yopulumutsira ndalama
female
Koma lachisanu sabata yatha, iwo anapita ku dziko la Democratic Republic of Congo DRC, kukakambirana ndi mtsogoleri wadzikolo, nkhani zokhudza chitetezo
Koma lachisanu sabata yatha, iwo anapita ku dziko la Dimokaratiki Ripabuliki ofu kongo (DI ARA SI), kukakambirana ndi mtsogoleri wadzikolo, nkhani zokhudza chitetezo
female
Mkulu wa bungwe la Centre for Social Accountability and Trasparency a Willy Kambwandira ati zomwe anachita a Chakwera sizikudabwitsa chifukwa awonetsa kuti alibe chidwi chosamalira chuma chadziko lino
Mkulu wa bungwe la Senta fo Sosho Akowuntabilite andi Tirasiparensi a Wile Kambwandira ati zomwe anachita a Chakwera sizikudabwitsa chifukwa awonetsa kuti alibe chidwi chosamalira chuma chadziko lino
female
Sitikudabwa ngakhale a Chakwera analonjeza kuti ayima kaye maulendo akunja, kuti ateteze ndalama akupitirizabe kuyenda
Sitikudabwa ngakhale a Chakwera analonjeza kuti ayima kaye maulendo akunja, kuti ateteze ndalama akupitirizabe kuyenda
female
Izi zachitsa kuti ngakhale mabungwe a boma azichitaso chimodzimodzi. Iwo adatero.
Izi zachitsa kuti ngakhale mabungwe a boma azichitaso chimodzimodzi. Iwo adatero.
female
A Kambwandira adati, polephera kutsata malamulo omwe adakoza yekha, mtsogoleri wa dzikolinoyu, wapereka chitsanzo choyipa.
A Kambwandira adati, polephera kutsata malamulo omwe adakoza yekha, mtsogoleri wa dzikolinoyu, wapereka chitsanzo choyipa.
female
Ngati mtsogoleri wadziko akuphwanya malamulo ake omwe, zikusonyeza kuti nkhani yoteteza chuma cha dzikolino, inali ya mchezochabe osati yeniyeni
Ngati mtsogoleri wadziko akuphwanya malamulo ake omwe, zikusonyeza kuti nkhani yoteteza chuma cha dzikolino, inali ya mchezochabe osati yeniyeni
female
Chifukwa choti a Malawi sakuchitapo kanthu a Chakwera akamawononga ndalama, sakuwawopaso, iwo adatero.
Chifukwa choti a Malawi sakuchitapo kanthu a Chakwera akamawononga ndalama, sakuwawopaso, iwo adatero.
female
Mtsogoleri wa bungwe la Centre for Human Rights and Rehabillitation, a Michael Kayiyatsa, anati popita kunja kwadzikolino, a Chakwera atayitsa anthu chikhulupiriro, pankhani yochepetsa kuwononga kwa ndalama
Mtsogoleri wa bungwe la Senta fo Humani Rayitsi andi Rihabilitashoni, a Mayikolo Kayiyatsa, anati popita kunja kwadzikolino, a Chakwera atayitsa anthu chikhulupiriro, pankhani yochepetsa kuwononga kwa ndalama
female
Kaya ulendo unali wofunikira kapena ayi, achotsabe chikhulupiriro cha a Malawi. Chimene a Chakwera adakachita ndi kutumiza nduna, mmalo mophwanya lamulo lawo lomwe. Iwo anatero.
Kaya ulendo unali wofunikira kapena ayi, achotsabe chikhulupiriro cha a Malawi. Chimene a Chakwera adakachita ndi kutumiza nduna, mmalo mophwanya lamulo lawo lomwe. Iwo anatero.
female
Nayeso kadawulo pazachuma ku sukulu ya ukachenjede ya Catholic University of Malawi, a Greenson Chijinthi, anati ulendowu, sunakwanilitse cholinga chopulumutsa ndalama zakunja.
Nayeso kadawulo pazachuma ku sukulu ya ukachenjede ya katholiki Univesite ofu Malawi, a Girinisoni Chijinthi, anati ulendowu, sunakwanilitse cholinga chopulumutsa ndalama zakunja.
female
Apapa tawononga ndalama zambiri zakunja, komaso ngati mtsogoleri wadziko akuyendayenda kunja, akuluakulu m’boma nawoso aziti nafeso titsatire zomwe mtsogoleri akuchita.
Apapa tawononga ndalama zambiri zakunja, komaso ngati mtsogoleri wadziko akuyendayenda kunja, akuluakulu m’boma nawoso aziti nafeso titsatire zomwe mtsogoleri akuchita.
female
Zikatere pamakhala chisokonezo chokhachokha, iwo anatero.
Zikatere pamakhala chisokonezo chokhachokha, iwo anatero.
female
Mneneri wa boma a Moses Kunkuyu, anapempha kuti atumiziridwe mafunso, koma anali asanayankhe, pamene timasindikiza nkhaniyi.
Mneneri wa boma a Mozesi Kunkuyu, anapempha kuti atumiziridwe mafunso, koma anali asanayankhe, pamene timasindikiza nkhaniyi.
female
Koma m’mbuyomu a Kunkuyu, anawuza News Paper ya Nation, kuti ulendowu unali wofunikira kwambiri.
Koma m’mbuyomu a Kunkuyu, anawuza Nyuzi Pepala ya Nashoni, kuti ulendowu unali wofunikira kwambiri.
female
Chifukwa anakambirana ndi mtsogoleri wadzikolo a Felix Chisekedi, nkhani zokhuza chitetezo.
Chifukwa anakambirana ndi mtsogoleri wadzikolo a Felikisi Chisekedi, nkhani zokhuza chitetezo.
female
Walira mvula waliraso matope, anthu amene amalakalaka atapeza chiphaso cha uzika, mwayi wawagwera, koma ayenera akhetse thukuta kuti izi zitheke.
Walira mvula waliraso matope, anthu amene amalakalaka atapeza chiphaso cha uzika, mwayi wawagwera, koma ayenera akhetse thukuta kuti izi zitheke.
female
Izi zikudza pamene nthambi yaboma yowona za kalembera wosiyanasiyana, ya National Registration Beureu
Izi zikudza pamene nthambi yaboma yowona za kalembera wosiyanasiyana, ya Nashonolo Rejisitireshoni Biyuro
female
NRB, yayamba kuyenda mzigawo, komwe akuthandiza anthu amene akufuna zitupa za uzika.
ENI ARA BI, yayamba kuyenda mzigawo, komwe akuthandiza anthu amene akufuna zitupa za uzika.
female
Kalemberayu akuchitika kuti amene akwanitsa zaka 16, apeze zitupa za unzika komaso kupereka mwayi kwa amene adataya zitupa
Kalemberayu akuchitika kuti amene akwanitsa zaka sikisitini, apeze zitupa za unzika komaso kupereka mwayi kwa amene adataya zitupa
female
Mwina kuwonongeka, kuti apeze zatsopano, komaso kulembetsa amene adatisiya, nthenda yakula ndi kutalika kwa malo okadulitsira chiphaso, zomwe anthu ambiri ati sakwanitsa
Mwina kuwonongeka, kuti apeze zatsopano, komaso kulembetsa amene adatisiya, nthenda yakula ndi kutalika kwa malo okadulitsira chiphaso, zomwe anthu ambiri ati sakwanitsa
female
Kutha ndalama kuti akapeze chitupa, ndondomekoyi yomwe yayamba m’maboma a kumwera, m’boma la Mzimba, Ntchisi, Ntcheu.
Kutha ndalama kuti akapeze chitupa, ndondomekoyi yomwe yayamba m’maboma a kumwera, m’boma la Mzimba, Ntchisi, Ntcheu.
female
Phalombe ndi Nsanje pa 13 January ikuyembekezeka kutha lero pa 27 January
Phalombe ndi Nsanje pa fetini Januware ikuyembekezeka kutha lero pa tuwente seveni Januware
female
Ku Ntcheu ndi Nsanje anthu ati akuyenda mtunda oposa ma Kilometre 50, kuti akapeze malo amene akuadulitsira chiphaso
Ku Ntcheu ndi Nsanje anthu ati akuyenda mtunda oposa ma Kilometre fifite, kuti akapeze malo amene akuadulitsira chiphaso
female
Anthu amene acheza ndi tamvani m’boma la Nsanje, ati mtima wafuna kukhala ndi chiphaso, koma thupi likunana kutero, chifukwa cha kutalirika kwa malo odulitsira chitupa.
Anthu amene acheza ndi tamvani m’boma la Nsanje, ati mtima wafuna kukhala ndi chiphaso, koma thupi likunana kutero, chifukwa cha kutalirika kwa malo odulitsira chitupa.
female
Mmodzi mwa anthuwo a Devis Moses Mtchola omwe amakhala ku Misavu mdera la T/A Tengani m’bomalo, ati anthu ambiri alibe mwayi wopeza chitupa cha uzika, chifukwa m’dera lawo mulibe malo olembetserako ziphasozi.
Mmodzi mwa anthuwo a Devisi Mozesi Mtchola omwe amakhala ku Misavu m'dera la Tiye Tengani m’bomalo, ati anthu ambiri alibe mwayi wopeza chitupa cha uzika, chifukwa m’dera lawo mulibe malo olembetserako ziphasozi.
female
Kuti akalembetse akuyenda mtunda wa utali, iwo adati kuno ngakhaleso ku Misavu, Million, Kawa, Kamanga, Bwangu, Nandilimbe
Kuti akalembetse akuyenda mtunda wa utali, iwo adati kuno ngakhaleso ku Misavu, Miliyoni, Kawa, Kamanga, Bwangu, Nandilimbe
female
Tikuyenera kupita ku Bangula kapena ku Mangoti kwa Sojini, komwe ndi ma Kilometre a pakatikati 37 ndi 42, kuti tikapeze chiphaso cha nzika
Tikuyenera kupita ku Bangula kapena ku Mangoti kwa Sojini, komwe ndi ma Kilomita a pakatikati sete seveni ndi fote thu, kuti tikapeze chiphaso cha nzika
female
Ulendowu timalipira 10,000 kwacha kupita kokha, ambiri tapanga chiganizo chosapitako, chifukwa ndife anthu wovutika, sitingapeze ndalama imeneyo, adatero
Ulendowu timalipira teni sawuzande kwacha kupita kokha, ambiri tapanga chiganizo chosapitako, chifukwa ndife anthu wovutika, sitingapeze ndalama imeneyo, adatero
female
A Mtchola ati atadandawula adawuzidwa kuti kwawoko kulibe magetsi, pomwe nthawi ya kalembera wa mavoti, pafupifupi dera lililonse kumakhala malo wolembetsera
A Mtchola ati atadandawula adawuzidwa kuti kwawoko kulibe magetsi, pomwe nthawi ya kalembera wa mavoti, pafupifupi dera lililonse kumakhala malo wolembetsera
female
Ndife wokhumudwa, siife tokha, azathu akwa Nthondo akuyenda ma kilometre oposa 30 kupita ku mpatsa.
Ndife wokhumudwa, siife tokha, azathu akwa Nthondo akuyenda ma kilomita oposa sete kupita ku mpatsa.
female
Pomwe ena ngati a Kunyamigeti, akutsetsereka kupita ku Mthawira, zomwe zapangitsa ambiri kuti asakhale ndi chidwi ndi ntchitoyi, adatero a Mtchola.
Pomwe ena ngati a Kunyamigeti, akutsetsereka kupita ku Mthawira, zomwe zapangitsa ambiri kuti asakhale ndi chidwi ndi ntchitoyi, adatero a Mtchola.
female
A Paul Malola ochokera m’dera la T/A Mulolo, ku Nsanje komweko, adati ndizokhumudwaitsa kuti Mlulolo yense bungwero layika malo atatu okha wolembetsera, omwe ndi Kalulu, Mbwazi ndi Sankhulani.
A Poo Malola ochokera m’dera la Tiye Mulolo, ku Nsanje komweko, adati ndizokhumudwaitsa kuti Mlulolo yense bungwero layika malo atatu okha wolembetsera, omwe ndi Kalulu, Mbwazi ndi Sankhulani.
female
Zomwe zikupereka chiopsyezo kwa anthu ochokere m’madera ngati Thamboni, Iron, Mchacha, Alfazema ndi ku Masenjere kuti sangakwanitse kulembetsa.
Zomwe zikupereka chiopsyezo kwa anthu ochokere m’madera ngati Thamboni, Ayironi, Mchacha, Alifazema ndi ku Masenjere kuti sangakwanitse kulembetsa.
female
A Malola adati akadakonda bungwero likadabwereka zipangizo za bungwe la chisankho la Malawi Electral Commision MEC, zomwe amapitanazo paliponse, potengera kufunikira kwa chiphaso chawunzika.
A Malola adati akadakonda bungwero likadabwereka zipangizo za bungwe la chisankho la Malawi Elekitiro Comisho (Meki), zomwe amapitanazo paliponse, potengera kufunikira kwa chiphaso chawunzika.
female
Kafukufuku wathu, akusonyeza kuti anthu omwe amakhalira ku mapiri monga Ching’oma, Bambala, Kavulathenga komaso Chimdzete,
Kafukufuku wathu, akusonyeza kuti anthu omwe amakhalira ku mapiri monga Ching’oma, Bambala, Kavulathenga komaso Chimdzete,
female
Akuyenda ndi kutsetsereka mapiri ndikufika pa school ya primary ya Mchere, zomwe achikulire sakukwanitsa, chifukwa chakutalika kwa mtunda.
Akuyenda ndi kutsetsereka mapiri ndikufika pa school ya pulayimale ya Mchere, zomwe achikulire sakukwanitsa, chifukwa chakutalika kwa mtunda.
female
Wapampando wa mabungwe omwe siaboma ku Nsanje a Mike Dansa, apempha bungwe la NRB, kuti lichite chilichonse chotheka, ndi kuwapatsa malo ena olembetsera ziphasozi anthuwa.
Wapampando wa mabungwe omwe siaboma ku Nsanje a Mayiki Dansa, apempha bungwe la ENI ARA BI, kuti lichite chilichonse chotheka, ndi kuwapatsa malo ena olembetsera ziphasozi anthuwa.
female
Chiphaso cha unzika mchawulere, ndiye palibe chifukwa choti anthu aziwonongera ndalama zoposa 20,000 kwacha, pofuna kukapangitsa chiphaso, uku ndikupherana ufulu.
Chiphaso cha unzika mchawulere, ndiye palibe chifukwa choti anthu aziwonongera ndalama zoposa tuwente sawuzande kwacha, pofuna kukapangitsa chiphaso, uku ndikupherana ufulu.
female
Ife tikufuna boma lipange monga momwe amachitira nthawi ya kalembera wa mavoti, powapatsa mwayi anthuwa, ndikuwafikira, cholinga choti alembedwe masiku omwe adayika asanathe.
Ife tikufuna boma lipange monga momwe amachitira nthawi ya kalembera wa mavoti, powapatsa mwayi anthuwa, ndikuwafikira, cholinga choti alembedwe masiku omwe adayika asanathe.
female
Iwo adati, chiphasochi nchofunika ndipo ambiri ziphaso zawo kumeneko, zidapita ndi madzi wosefukira. Chiphaso cha unzika ndi moyo.
Iwo adati, chiphasochi nchofunika ndipo ambiri ziphaso zawo kumeneko, zidapita ndi madzi wosefukira. Chiphaso cha unzika ndi moyo.
female
Popanda chimenecho, munthu sungakhale ndi mtendere popeza uzitengedwa ngati ndiwe obwera. Boma yesetsani kutithandiza
Popanda chimenecho, munthu sungakhale ndi mtendere popeza uzitengedwa ngati ndiwe obwera. Boma yesetsani kutithandiza
female
Paja kuno anthu ambiri anataya ziphaso zawo ndi a namondwe omwe anabwera pakatipa ngati Anna, Gombe ndi Freddy, anatero a Dansa.
Paja kuno anthu ambiri anataya ziphaso zawo ndi a namondwe omwe anabwera pakatipa ngati Ana, Gombe ndi Furede, anatero a Dansa.
female
Izi ziliyapo, madzi afika mkhosi ku Ntcheu, komwe phungu wina kumeneko, Wayamba kutumiza galimoto, kuti ikatenge anthu m’dera lake lokha, kuti akapeze chiphaso, atawona kutalika kwa mtunda.
Izi ziliyapo, madzi afika mkhosi ku Ntcheu, komwe phungu wina kumeneko, Wayamba kutumiza galimoto, kuti ikatenge anthu m’dera lake lokha, kuti akapeze chiphaso, atawona kutalika kwa mtunda.
female
A Dickso Austin, okhala ku Gawaza kwa T/A Phambala adati komwe NRB ikudulitsa ziphaso ndi kwa Senzani komwe ndi mtunda oposa ma kilometre 50, kupita kokha.
A Dikisoni Ositini, okhala ku Gawaza kwa Tiye Phambala adati komwe eni ara bi ikudulitsa ziphaso ndi kwa Senzani komwe ndi mtunda oposa ma kilomita fifite, kupita kokha.
female
Galimoto sizifika kuno, yankho ndi njingayamoto basi, ndiye kupita kokha ndi 15,000-kwacha kuti ukafike ku mnsewu watala, komwe ungakapeze bus.
Galimoto sizifika kuno, yankho ndi njingayamoto basi, ndiye kupita kokha ndi fifitini sawuzande kwacha kuti ukafike ku mnsewu watala, komwe ungakapeze Basi.
female
Ndiye pobwera, uyeneraso upeze ndalama, tizitenga kuti ndi njalayi? Adadabwa a Austin.
Ndiye pobwera, uyeneraso upeze ndalama, tizitenga kuti ndi njalayi? Adadabwa a Ositini.
female
A Joyce Magugu, a m’mudzi mwa Njonjo, T/A Masasa, adati kumeneko kuli anthu ambiri ofuna kupeza ziphaso, koma vuto ndi mtunda omwe akuyenda.
A Joyisi Magugu, a m’mudzi mwa Njonjo, Tiye Masasa, adati kumeneko kuli anthu ambiri ofuna kupeza ziphaso, koma vuto ndi mtunda omwe akuyenda.
female
Kukafika komwe akudulitsako ndi ma kilometre 15, tikapita ndiye kuti kubwera ndi usiku, chifukwa kukumakhalaso mzere wawukulu, kuti anthu athandizidwe.
Kukafika komwe akudulitsako ndi ma kilomita fifitini, tikapita ndiye kuti kubwera ndi usiku, chifukwa kukumakhalaso mzere wawukulu, kuti anthu athandizidwe.
female
Ndibwino akadawonjezera masiku, chifukwa kunoko vuto lomwe lakulaso ndi Network, yomwe sikudalirika, adatero.
Ndibwino akadawonjezera masiku, chifukwa kunoko vuto lomwe lakulaso ndi Netiweki, yomwe sikudalirika, adatero.
female
Ndipo polankhula pa school ya secondary ya Ntowe, phungu wa kunyumba ya malamulo wadera la Nsanje Lalanje, mayi Gladys Ganda, adamema anthu m’bomalo, kuti akalembetse ziphaso za uzika.
Ndipo polankhula pa sukulu ya sekondale ya Ntowe, phungu wa kunyumba ya malamulo wadera la Nsanje Lalanje, mayi Giladesi Ganda, adamema anthu m’bomalo, kuti akalembetse ziphaso za uzika.
female
A Ganda adati kufunikira kwa ziphasozi nkwakukulu, ponena kuti, ziwathandizira nthawi yopeza zipangizo zotsika mtengo, kukhala umboni wotsekulira ma book aku bank.
A Ganda adati kufunikira kwa ziphasozi nkwakukulu, ponena kuti, ziwathandizira nthawi yopeza zipangizo zotsika mtengo, kukhala umboni wotsekulira ma buku aku banki.
female
Kupeza mwayi wopangitsa zitupa zoyendera komaso kudzakhala ndi mwayiwolembetsa mkawundula wa chisankho kuti adzathe ku vota pa 16 September, chaka chamawa.
Kupeza mwayi wopangitsa zitupa zoyendera komaso kudzakhala ndi mwayiwolembetsa mkawundula wa chisankho kuti adzathe ku vota pa sikisitini Seputembala, chaka chamawa.
female
Komabe phunguyu yemwe anaperekezedwa ndi govenor wa chipani cha Democratic Progressive Party DPP ku chigawo cha kumwera a Thomson Kamangira.
Komabe phunguyu yemwe anaperekezedwa ndi gavanala wa chipani cha Dimokiratiki Pulogiresivi Pate DiPiPi ku chigawo cha kumwera a Thomusoni Kamangira.
female
Ndipo amayendera malo ngati Sojini, Bangula, Phokera, Pagala pa boma la Nsanje, Fargo ndi Ntowe, anadandawula ndi momwe ntchitoyi ikuyendera.
Ndipo amayendera malo ngati Sojini, Bangula, Phokera, Pagala pa boma la Nsanje, Fago ndi Ntowe, anadandawula ndi momwe ntchitoyi ikuyendera.
female
Ponena kuti ogwira ntchito ndiwochepa ndipo anapempha nthambi ya NRB kuti iwonjezere masiku ogwira ntchitoyi.
Ponena kuti ogwira ntchito ndiwochepa ndipo anapempha nthambi ya eni ara bi kuti iwonjezere masiku ogwira ntchitoyi.
female
Poyankhapo mlembi wa mkulu ku NRB a Mphatso Sambo, anati zose zikuyenda bwino popeza anthu akulembetsa ziphasozi.
Poyankhapo mlembi wa mkulu ku eni ara bi a Mphatso Sambo, anati zose zikuyenda bwino popeza anthu akulembetsa ziphasozi.
female
Iwo anati tili m’gawo lachisanu ya ntchitoyi, yomwe tikugwira m’maboma a Nsanje, Phalombe, Ntchisi ndi ku mpoto kwa boma la Mzimba.
Iwo anati tili m’gawo lachisanu ya ntchitoyi, yomwe tikugwira m’maboma a Nsanje, Phalombe, Ntchisi ndi ku mpoto kwa boma la Mzimba.
femalo
Ntchitoyi, tidayamba pa 13 January ndipo idzatha pa 27 January, 2024, awa ndi masiku 15, ndipo tikulembera ziphaso za unzika, ziphaso za omwe anamwalira, komaso ziphaso zamabanja.
Ntchitoyi, tidayamba pa setini Januware ndipo idzatha pa tuwente seveni Januware, tewente tuwente folo, awa ndi masiku fifitini, ndipo tikulembera ziphaso za unzika, ziphaso za omwe anamwalira, komaso ziphaso zamabanja.
female
Iwo adati, m’boma momwe tikugwira, tinatengako magawo 25, pa 100 aliwonse, amene ali m’boma ndipo amasankhidwa mogwirizana ndi a khonsolo, ndipo pamakhala ndi malo akulu amodzi.
Iwo adati, m’boma momwe tikugwira, tinatengako magawo tuwente fayife, pa wani handirede aliwonse, amene ali m’boma ndipo amasankhidwa mogwirizana ndi a khonsolo, ndipo pamakhala ndi malo akulu amodzi.
female
Tikuunguza momwe ntchitoyi yayendera, ndipo tikaona kuti nkofunika kuwonjezera masiku akalemberayu, tichita motero, mukudziwa a Phalomba ndi Nsanje, zitupa zambiri zidapita ndi madzi.
Tikuunguza momwe ntchitoyi yayendera, ndipo tikaona kuti nkofunika kuwonjezera masiku akalemberayu, tichita motero, mukudziwa a Phalomba ndi Nsanje, zitupa zambiri zidapita ndi madzi.
female
Nthawi ya namondwe wa Freddy adatero iwo, ndipo adawonjeza kuti akatseka kalembera alipoyu, anthu akhoza kupita ku ma office awo pa boma kapena ku Post Office.
Nthawi ya namondwe wa Furede adatero iwo, ndipo adawonjeza kuti akatseka kalembera alipoyu, anthu akhoza kupita ku ma ofesi awo pa boma kapena ku Positi Ofesi.
female