audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
A Chithere ati, anthu omwe agwidwa poganiziridwa kutenga gawo pakuphedwa kwa abambowo, ndi a Gift Manuel azaka 37.
A Chithere ati, anthu omwe agwidwa poganiziridwa kutenga gawo pakuphedwa kwa abambowo, ndi a Gifiti Manuwelo azaka sete seveni.
female
A Nedson Taulo azaka 50, a Shadreck Manuel azaka 52, a Thokozani Semion azaka 26, a Billy Yamikani a zaka 30, komaso a John Malichi azaka 32
A Nedisoni Tawulo azaka fifite, a Shadireki Manuwelo azaka fifite-thu, a Thokozani Simiyoni azaka tuwente sikisi, a Bile Yamikani a zaka sete, komaso a Joni Malichi azaka sete-thu
female
Iwo ati, anthu onsewa amachokera m’mudzi mwa Mtiza, kwa mfumu yayikulu Mabuka ku Mulanje, ndipo akuyankha mlandu wakupha kubwalo la milandu posachedwapa.
Iwo ati, anthu onsewa amachokera m’mudzi mwa Mtiza, kwa mfumu yayikulu Mabuka ku Mulanje, ndipo akuyankha mlandu wakupha kubwalo la milandu posachedwapa.
female
A bamboo omwe adaphedwawo ndi a Willy Manyowa, omwe zakazawo sizikudziwika koma ndi a chikulire.
A bamboo omwe adaphedwawo ndi a Wile Manyowa, omwe zakazawo sizikudziwika koma ndi a chikulire.
female
A John Maudzu azaka 31, a Madalitso Mailosi azaka 25, pomweso winayo sakudziwika.
A Joni Maudzu azaka sete-wani, a Madalitso Mayilosi azaka tuwente-fayifi, pomweso winayo sakudziwika.
female
A Chimthere ati mnyengo yazisangalalo yomwe yafikayi, oganiziridwa milandu amakhala ochuluka, ndipo apempha anthu kuti akagwira munthu woganiziridwa azipitanaye ku Police.
A Chimthere ati mnyengo yazisangalalo yomwe yafikayi, oganiziridwa milandu amakhala ochuluka, ndipo apempha anthu kuti akagwira munthu woganiziridwa azipitanaye ku Polisi.
female
Kuti a Police apange kafukufuku wawo, nkuyendetsa nkhaniyo, motsata malamulo.
Kuti a Polisi apange kafukufuku wawo, nkuyendetsa nkhaniyo, motsata malamulo.
female
Mayi wazaka 19 wadzipha ku Kasungu, atazindikira kuti mwamuna yemwe adakwatirana naye, pokhulupirira kuti banja lake loyamba lidatha ndi mkaziwake, akupangabe chikwati ndi mkaziyo mwa m’seri.
Mayi wazaka nayintini wadzipha ku Kasungu, atazindikira kuti mwamuna yemwe adakwatirana naye, pokhulupirira kuti banja lake loyamba lidatha ndi mkaziwake, akupangabe chikwati ndi mkaziyo mwa m’seri.
female
Izi zachitika m’mudzi mwa Matatiyo, mfumu yayikulu Magwazu m’bomalo, komwe mayi Mtisunge Makwinja, adakakwatiwa ndi mamuna yemwe adamuuza kuti banja lake loyamba lidatha ndi mkaziwake.
Izi zachitika m’mudzi mwa Matatiyo, mfumu yayikulu Magwazu m’bomalo, komwe mayi Mtisunge Makwinja, adakakwatiwa ndi mamuna yemwe adamuuza kuti banja lake loyamba lidatha ndi mkaziwake.
female
Wachiwiri kwa m’neneri wa police ya Kasungu a Miracle Nkozi, ati banja latsopanolo litayamba, Makwinja adazindikira kuti mamuna wakeyo, akuzemberanabe ndi mkazi wake wakale.
Wachiwiri kwa m’neneri wa polisi ya Kasungu a Mirako Nkozi, ati banja latsopanolo litayamba, Makwinja adazindikira kuti mamuna wakeyo, akuzemberanabe ndi mkazi wake wakale.
female
Ndipo iye adachenjeza mamunayo kuti asiye, zikuoneka kuti mamunayo sadafune kusiya kuyenda ndi mkazi wake woyambayo.
Ndipo iye adachenjeza mamunayo kuti asiye, zikuoneka kuti mamunayo sadafune kusiya kuyenda ndi mkazi wake woyambayo.
female
Mpaka pa 18 November, kudabuka mkangano pakati pa mamunayo ndi Makwinja pankhaniyo. Atero a Nkozi.
Mpaka pa eyitini Novembala, kudabuka mkangano pakati pa mamunayo ndi Makwinja pankhaniyo. Atero a Nkozi.
female
Iwo ati pa 19 November 2023, banjalo lidapita kumunda limodzi, koma malemu Makwinja, adanyamukako changu.
Iwo ati pa nayintini Novembala tuwente tuwente-firi, banjalo lidapita kumunda limodzi, koma malemu Makwinja, adanyamukako changu.
female
Kusiya bamboyo akugwirabe ntchito kumundako, ndipo iye atafika kunyumba adamwa mankhwala omwe sadadziwike.
Kusiya bamboyo akugwirabe ntchito kumundako, ndipo iye atafika kunyumba adamwa mankhwala omwe sadadziwike.
female
A Nkozi ati, anthu achifundo adatengera Makwinja ku chipatala cha Kasungu, komwe adafikira kuuzidwa kuti mayiyo adali atamwalirakale, ndipo chomupha chidali mankhwala omwe akuganiziridwa kuti adamwawo.

Malingana ndi a Nkozi, malemu a Makwinja, amachokera m’mudzi mwa Katema kwa mfumu yayikulu Kaomba, m’boma la Kasungu lomwelo.
Malingana ndi a Nkozi, malemu a Makwinja, amachokera m’mudzi mwa Katema kwa mfumu yayikulu Kaomba, m’boma la Kasungu lomwelo.
female
Gawo 17, lamalamulo adzikolino, lokhudzana ndi mabanja komaso kutha kwa mabanjawo, limati polowa m’banja lodziwika ku boma
Gawo seventini, lamalamulo adzikolino, lokhudzana ndi mabanja komaso kutha kwa mabanjawo, limati polowa m’banja lodziwika ku boma
female
Munthu amayenera kuwulura chilungamo ngati Sali pabanja, ndipo gawo 51 lamalamulo omwewo, limati munthu yemwe walowa m’banja alikale pa banja lina koma sadawulure.
Munthu amayenera kuwulura chilungamo ngati Sali pabanja, ndipo gawo fifite-wani lamalamulo omwewo, limati munthu yemwe walowa m’banja alikale pa banja lina koma sadawulure.
female
Akapezeka wolakwa, amayenera kulipira 100,000 kwacha, kapena kukasewenza, zaka 5.
Akapezeka wolakwa, amayenera kulipira wani handirede sauzande kwacha, kapena kukasewenza, zaka fayifi.
female
Izi zili yapa, phungu wa kum’mwera m’boma la Lilongwe, a Peter Dimba, a Malawi Congress Party, M.C.P, apempha boma kuti lichotse mlandu wa anthu ofuna kudzipha.
Izi zili yapa, phungu wa kum’mwera m’boma la Lilongwe, a Pita Dimba, a Malawi kongiresi Pate, EMUSIPI, apempha boma kuti lichotse mlandu wa anthu ofuna kudzipha.
female
Chifukwa nthawi zambiri, anthu ofika apa amakhala asakuganiza moyenera, ndipo akufunika thandizo lina, osakhala chilango.
Chifukwa nthawi zambiri, anthu ofika apa amakhala asakuganiza moyenera, ndipo akufunika thandizo lina, osakhala chilango.
female
Polankhula mnyumbayo, popereka maganizo awo pa report la momwe kaganizidwe ka gwiro kalili m’dziko muno, a Dimba anati nthawi zambiri anthu amafuna kuzipha
Polankhula mnyumbayo, popereka maganizo awo pa report la momwe kaganizidwe ka gwiro kalili m’dziko muno, a Dimba anati nthawi zambiri anthu amafuna kuzipha
female
kaamba kazifukwa zoti kuziwunikira bwino. Kuti munthu afike poganiza zozipha, ndiyekuti zinthu zathina osati masewera.
kaamba kazifukwa zoti kuziwunikira bwino. Kuti munthu afike poganiza zozipha, ndiyekuti zinthu zathina osati masewera.
female
kuti anthu ofuna kuzipha azimangidwa sizitithandiza adatero iwo. Theka loyamba la chaka chino, anthu 256 adazipha mdziko muno.
kuti anthu ofuna kuzipha azimangidwa sizitithandiza adatero iwo. Theka loyamba la chaka chino, anthu thu handirede andi fifite-sikisi adazipha mdziko muno.
female
poyerekeza ndi 135 chaka chatha. Mchitidwe wogona ndi ana ukukula kwambiri
poyerekeza ndi wani sete-fayifi chaka chatha. Mchitidwe wogona ndi ana ukukula kwambiri
female
pamene bwalo lina ku Zomba sabata yangothayi, lidagamula kuti mphunzitsi wina ndi wosalakwa pa mlandu wogwiririra mwana wophunzira pa sukulu ya zobwe ku Chingale m’bomalo.
pamene bwalo lina ku Zomba sabata yangothayi, lidagamula kuti mphunzitsi wina ndi wosalakwa pa mlandu wogwiririra mwana wophunzira pa sukulu ya zobwe ku Chingale m’bomalo.
female
Bwalo lina la mlandu m’boma la Phalombe, lagamula bambo wina wa zaka 45 kukaseweza zaka 12 ku ndende pogona ndi mwana wa zaka 15
Bwalo lina la mlandu m’boma la Phalombe, lagamula bambo wina wa zaka fotr-fayifi kukaseweza zaka thuwelofu ku ndende pogona ndi mwana wa zaka fifitini
female
Zigamulo ziwirizo dzadza musabata imene apolice alengeza kuti, chiwerengero cha milandu yokhudza kugwiririra ana chinafika pa 1000.
zigamulo ziwirizo dzadza musabata imene apolisi alengeza kuti, chiwerengero cha milandu yokhudza kugwiririra ana chinafika pa wani sauzande.
female
A police atalengeza kukwera kwa milandu yokhudza kugona ndi ana, m'modzi mwa oyimira anthu pamilandu yemwenso ndi womenyera ufulu wa ana,
zigamulo ziwirizo dzadza musabata imene apolice alengeza kuti, chiwerengero cha milandu yokhudza kugwiririra ana chinafika pa 1000.
female
A Lectious Kamangira, adati kugona ndi ana kumakula makamaka kaamba kousanza mtima.
A Lekishiyasi Kamangira, adati kugona ndi ana kumakula makamaka kaamba kousanza mtima.
female
Boma likuyenra kukhazikitsa njira zabwino zoteteza atsina ku mchitidwewu, komanso makolo ayenera kuteteza anawo
Boma likuyenra kukhazikitsa njira zabwino zoteteza atsina ku mchitidwewu, komanso makolo ayenera kuteteza anawo
female
Nzachisoni kuti ambiri mwa atsikana amagwiriridwa nda atate, malume, achimwene, asuweni ngakhalenso anzawo amene amayenera kuwateteza. Anatero a Kamangira
Nzachisoni kuti ambiri mwa atsikana amagwiriridwa nda atate, malume, achimwene, asuweni ngakhalenso anzawo amene amayenera kuwateteza. Anatero a Kamangira
female
Nkhani ya ku Zomba ikuti, bwalo la magestrate mzindawo, idapeza Chisomo Franscico Gomani wosalakwa pamulandu womuganizira kuti adagonana ndi mwana
Nkhani ya ku Zomba ikuti, bwalo la majisitireti mzindawo, idapeza Chisomo Furansisiko Gomani wosalakwa pamulandu womuganizira kuti adagonana ndi mwana
female
Malingana ndi zolembedwa pa tsamba la facebook la nthambi yaboma yoyimira oganiziridwa mwa ulele ya Legal Aid Beaural, a Gomani adamangidwa ndi police ya Chingale pa 27, October 2023.
Malingana ndi zolembedwa pa tsamba la fesibuku la nthambi yaboma yoyimira oganiziridwa mwa ulele ya Ligo Edi Biyuro, a Gomani adamangidwa ndi polisi ya Chingale pa tuwente-seveni, Okotobala, tuwente tuwente firi.
FEMALE
Ku bwalo la milandu woganiziridwawo adaukana mlanduwu, ndipo mbali ya boma idabweretsa mboni zitatu; mayi amwayu, mwanayu komanso kadaulo wa zachipatala
Ku bwalo la milandu woganiziridwawo adaukana mlanduwu, ndipo mbali ya boma idabweretsa mboni zitatu; mayi amwayu, mwanayu komanso kadaulo wa zachipatala
female
Mu umboni wawo mayi a mwanayo, adauza bwalolo nchemali wawo adabwera nkati mwa usiku kudzauza kuti adawona amuna awowo ali matimati ndi mwanayo mnyumba ina.
Mu umboni wawo mayi a mwanayo, adauza bwalolo nchemali wawo adabwera nkati mwa usiku kudzauza kuti adawona amuna awowo ali matimati ndi mwanayo mnyumba ina.
female
mayiyo adawonjeza kuti atapita kunyumbayo adawapezadi awiriwo koma mwanayo adathawa. Iwo adati pamalopo adapezapo condom imene idali ndi magazi
mayiyo adawonjeza kuti atapita kunyumbayo adawapezadi awiriwo koma mwanayo adathawa. Iwo adati pamalopo adapezapo kondomu imene idali ndi magazi
female
Ndipo mu umboni wawo wachipatala a Cathreen Maganizo adati atamuyeza mwanayo adapeza kuti adagonanapo ndi mwamuna kangapo konse.
Ndipo mu umboni wawo wachipatala a Cathreen Maganizo adati atamuyeza mwanayo adapeza kuti adagonanapo ndi mwamuna kangapo konse.
female
Kumbali yake, mwanayo adauza bwalo kuti adapita ku nyumba kwa a Gomani limozdi ndi nzake kuti akathandize kuchonga mayeso.
Kumbali yake, mwanayo adauza bwalo kuti adapita ku nyumba kwa a Gomani limozdi ndi nzake kuti akathandize kuchonga mayeso
female
Koma sadanene kalikonse kokhudza nkhani imene a police adawaitanira kuti akachitire umboni. Chidatero chikalatacho.
Koma sadanene kalikonse kokhudza nkhani imene a polisi adawaitanira kuti akachitire umboni. Chidatero chikalatacho.
female
umboni utaperekedwa, oyimira a Gomani kuchokera ku labu a Harneck Ching'anda, adatsindikiza kuti oganiziridwayo alimbe mulandu woti ayankhe chifukwa umboni womwe bwalo lidapatsidwa sudali wogwira mtima.
umboni utaperekedwa, oyimira a Gomani kuchokera ku labu a Harineki Ching'anda, adatsindikiza kuti oganiziridwayo alimbe mulandu woti ayankhe chifukwa umboni womwe bwalo lidapatsidwa sudali wogwira mtima.
female
Iwo adapitirizanso kuti mayi wamwanayo, adabwera ndi umboni womwe unali mphekesera chifukwa condom imene adatchulayo sanabwerenayo komanso mwanayo sadauze bwalo kuti nkhaniyo ndi yowona.
Iwo adapitirizanso kuti mayi wamwanayo, adabwera ndi umboni womwe unali mphekesera chifukwa kondomu imene adatchulayo sanabwerenayo komanso mwanayo sadauze bwalo kuti nkhaniyo ndi yowona.
female
Chigamulo chake a magestrate wa a Martin Chikofya, anagwirizana ndi LABU kuti ambali ya boma sanabwere ndi umboni wokwanira wotsimikiza kuti Gomani anagonana ndi mwana
Chigamulo chake a majisitiretiwa a Matini Chikofya, anagwirizana ndi LABU kuti ambali ya boma sanabwere ndi umboni wokwanira wotsimikiza kuti Gomani anagonana ndi mwana
female
Bwalolo lidawonanso kuti umboni unali wosakwanira komanso wosadalilika kuti mpaka munthu amangidwe.
Bwalolo lidawonanso kuti umboni unali wosakwanira komanso wosadalilika kuti mpaka munthu amangidwe.
female
Kotero bwalo lidapeza mphinzitsiyo kuti alibe mlandu kuti ayankhe malingana ndi zomwe amaganiziridwa.
Kotero bwalo lidapeza mphinzitsiyo kuti alibe mlandu kuti ayankhe malingana ndi zomwe amaganiziridwa.
female
Izi zili apo, bwalo la milandu ku Phalombe lagamula a Alfred Kamoto wa zaka 45 kuti akaseweze zaka 12 atapezeka wolakwa pogona ndi mwana wa zaka 15
Izi zili apo, bwalo la milandu ku Phalombe lagamula a Alafuredi Kamoto wa zaka fote fayifi kuti akaseweze zaka thuwelofu atapezeka wolakwa pogona ndi mwana wa zaka fifitini.
female
Mneneri wa police ya bomalo, a Jimmy Kapanja adati bamboyo wakhala akugona ndi mwanayo pakati pa November ndi mwezi uno.
Mneneri wa polisi ya bomalo, a Jime Kapanja adati bamboyo wakhala akugona ndi mwanayo pakati pa Novembala ndi mwezi uno.
female
Ndipo izi zidaululika pomwe mkuluyo akanena kuti mwanayo wamubera ufa, a Kapanja adati.
Ndipo izi zidaululika pomwe mkuluyo akanena kuti mwanayo wamubera ufa, a Kapanja adati.
female
maiy amwanayo atafunsa chifukwa chimene adabera ufa, adaulula kuti Kamoto adalephera kukwaniritsa zimene adalonjeza
maiy amwanayo atafunsa chifukwa chimene adabera ufa, adaulula kuti Kamoto adalephera kukwaniritsa zimene adalonjeza
female
Ndipo adapempha woweruza kuti apereke chilango chocheperako chifukwa ndi mutu wa banja lake
Ndipo adapempha woweruza kuti apereke chilango chocheperako chifukwa ndi mutu wa banja lake
female
Iwo adawonjeza kuti woyimira boma adati woweruza asamvere izi chifukwa kugona ndi mwana ndi mlandu waukulu ndipo a Leornard Mtosa adapereka chilangocho kwa bamboyo
Iwo adawonjeza kuti woyimira boma adati woweruza asamvere izi chifukwa kugona ndi mwana ndi mlandu waukulu ndipo a Lenadi Mtosa adapereka chilangocho kwa bamboyo
female
Malinga ndi mkulu wa bungwe lowona za ufulu wa ana la YUNECO, a Mc Ben Mkandawire adati kupsyolera mu njira yoyimba mafoni ya tithandizane help line, amalandira nkhani 5 kapena 6 zokhudza ana amene agonedwa
Malinga ndi mkulu wa bungwe lowona za ufulu wa ana la YUNECO, a Maki Beni Mkandawire adati kupsyolera mu njira yoyimba mafoni ya tithandizane helepu layini, amalandira nkhani fayifi kapena sikisi zokhudza ana amene agonedwa
female
Awa ndi ana amene amapereka malipoti awo, nanga amene nkhani zawo zimangothera mu mtima? pakuyenera kukhala njira zotetezera anawa. Adatero a Mkandawire
Awa ndi ana amene amapereka malipoti awo, nanga amene nkhani zawo zimangothera mu mtima? pakuyenera kukhala njira zotetezera anawa. Adatero a Mkandawire
female
Kutentha kwa mnanu kunkira. Nthambi ya zanyengo ya Department of Climate Change and Metiological Services yati kutentha kwa mnanu komwe kwakhala kukuwoneka madera ambiri,
Kutentha kwa mnanu kunkira. Nthambi ya zanyengo ya Dipatimenti ofu kilayimeti Chanji and Metiyolojiko Sevisesi yati kutentha kwa mnanu komwe kwakhala kukuwoneka madera ambiri.
female
Kunkira mpakana sabata ikudzayi. Mkulu wa nthambiyo, a Lucy Mtiratira, ati pachifukwachi mbiyang'ambe zichepetse kamwedwe ka bibida chifukwa sagwirizana nkutentha ndipo akhodza kuwapha mosavuta.
Kunkira mpakana sabata ikudzayi. Mkulu wa nthambiyo, a Luse Mtiratira, ati pachifukwachi mbiyang'ambe zichepetse kamwedwe ka bibida chifukwa sagwirizana nkutentha ndipo akhodza kuwapha mosavuta.
female
Nthambi ya za umoyo yalangiza anthu kupewa mowa. Chakumwa cha ukali chimayamwa madzi mthupi. Ndiye mthupi mopanda madzi nkutentha koonjeza sizigwirizana.
Nthambi ya za umoyo yalangiza anthu kupewa mowa. Chakumwa cha ukali chimayamwa madzi mthupi. Ndiye mthupi mopanda madzi nkutentha koonjeza sizigwirizana.
female
chifukwa thupi limafuna madzi kuti zambiri zizigwira ntchito. Atero Mtiratira.
chifukwa thupi limafuna madzi kuti zambiri zizigwira ntchito. Atero Mtiratira.
female
A Mtiratira ati kalosera sakuona kusintha kulikonse kwa nyengo yotenthayi nsanga, kotero anthu azionetsetsa kuti akumwa madzi ochuluka pa tsiku kuti m'matupi mwawo azikhalamo okwanira.
A Mtiratira ati kalosera sakuona kusintha kulikonse kwa nyengo yotenthayi nsanga, kotero anthu azionetsetsa kuti akumwa madzi ochuluka pa tsiku kuti m'matupi mwawo azikhalamo okwanira.
female
iwo atinso anthu achepetse kukhala pa dzuwa nthawi yayitali komanso kuti poyenda aziyesetsa kufunda mwafuli, ndipo pakavalidwe, ati kuvala mwa ulingawombe kukhodza kuonjezera chiwopsezo kwa munthu.

Magulu ena monga ana ndi okalamba aziyang'aniridwa bwino pa nyengo imeneyi chifukwa ndiwo ali pachiopsezo chachikulu ku nyengo yotentha mowonjezayi, iwo adatero.
Magulu ena monga ana ndi okalamba aziyang'aniridwa bwino pa nyengo imeneyi chifukwa ndiwo ali pachiopsezo chachikulu ku nyengo yotentha mowonjezayi, iwo adatero.
female
Malingana ndi chikalata chomwe nthambiyo idatulutsa cholotsera nyengo, madera akuchigwa cha shire ndiwo atentha kwambiri kumafika 42 degree celsius.
Malingana ndi chikalata chomwe nthambiyo idatulutsa cholotsera nyengo, madera akuchigwa cha shire ndiwo atentha kwambiri kumafika fote-thu digiri selishasi.
female
Motsatana ndi madera a mphepete mwa nyanja omwe azifika 38 degree celsius ndipo madera ana azifika 36 degree celsius.
Motsatana ndi madera a mphepete mwa nyanja omwe azifika set-eyiti digiri selishasi celsius ndipo madera ana azifikasete-sikisi digiri selishasi.
female
Kutenthaku komwe sikunasiye dera, kukumanyanya masana kuyambira mma 11 koloko mpakana mma 3 koloko, nthawi yomwe anthu amakhala otanganidwa ndi ntchiti zosiyanasiyana.
Kutenthaku komwe sikunasiye dera, kukumanyanya masana kuyambira mma leveni koloko mpakana mma firi koloko, nthawi yomwe anthu amakhala otanganidwa ndi ntchiti zosiyanasiyana.
female
kadaulo pa zachilengedwe, a Mathews Malata, adachenjeza kuti momwe anthu akuonongera chilengedwe monga nkhalango komanso kusasamala katayidwe kama plastic
kadaulo pa zachilengedwe, a Mafiyuzi Malata, adachenjeza kuti momwe anthu akuonongera chilengedwe monga nkhalango komanso kusasamala katayidwe kama pulasitiki
female
ndi zinthu zomwe siziwola, asamadabwe akamakumana ndi nyengo zodabwitsa. Nyengo zodabwitsa tikukonza tokha chifukwa chosasamala chilengedwe.
ndi zinthu zomwe siziwola, asamadabwe akamakumana ndi nyengo zodabwitsa. Nyengo zodabwitsa tikukonza tokha chifukwa chosasamala chilengedwe.
female
Nkhani ya kusintha kwa nyengo ikulengezedwa tsiku ndi tsiku ndipo zochititsa izi ndi zotsatira zake zikulengezedwa koma sitikusintha. adaterpo a Malata
Nkhani ya kusintha kwa nyengo ikulengezedwa tsiku ndi tsiku ndipo zochititsa izi ndi zotsatira zake zikulengezedwa koma sitikusintha. adaterpo a Malata
female
Chiwanda chophana chavuta. chiwanda chachilendo chophana mmabanja chalowerera, moti mwezi umodzi wokha bambo wina ku Zomba adapha mkazi wake
Chiwanda chophana chavuta. chiwanda chachilendo chophana mmabanja chalowerera, moti mwezi umodzi wokha bambo wina ku Zomba adapha mkazi wake
female
Banja lina ku Chiradzulu lidapha mwana wawo, pomwe mwana wa zaka 15 ku Chitipa adapha agogo ake
Banja lina ku Chiradzulu lidapha mwana wawo, pomwe mwana wa zaka fifitini ku Chitipa adapha agogo ake
female
Lachitatu pa 10 October 2023, bambo wa zaka 27 a Duby Mkwinjiri adapha mkazi wawo wa zaka 20.
Lachitatu pa teni Okotobalatuwente tuwente-firi, bambo wa zaka tuwente-seveni a Duby Mkwinjiri adapha mkazi wawo wa zaka tuwente.
female
Ndiwuzayani Pemphani m'boma la zomba pankhani yokhudzana ndi masalamusi omwe bamboyo amkafuna kuchita.
Ndiwuzayani Pemphani m'boma la zomba pankhani yokhudzana ndi masalamusi omwe bamboyo amkafuna kuchita.
female
Mneneri wa police mboma la Zomba, mayi Patricia Sipiriyano, atsimikiza kuti akusunga mchitokosi bamboyo yemwe kafukufulku akatha, akayankhe mlandu wakupha
Mneneri wa polisi mboma la Zomba, mayi Patirisha Sipiriyano, atsimikiza kuti akusunga mchitokosi bamboyo yemwe kafukufulku akatha, akayankhe mlandu wakupha
female
Tidalandira lipoti loti bamboyo yemwe amakhala mmudzi mwa Mowa kwa Jali, wapha mkazi wake. Ndipo titapita mmudzimo,
Tidalandira lipoti loti bamboyo yemwe amakhala mmudzi mwa Mowa kwa Jali, wapha mkazi wake. Ndipo titapita mmudzimo,
female
tidapezadi kuti mkaziyi ali thapsa mmagazi ake omwe atabayidwabayidwa, atero a Sipiriyano.
tidapezadi kuti mkaziyi ali thapsa mmagazi ake omwe atabayidwabayidwa, atero a Sipiriyano.
female
koma munthu yemwe adatitsina khutu za nkhaniyi, adati bamboyo adakatenga mankhwala oti alemere ndipo adauzidwa kuti akwilire mankhwalawo mnyumba kuti aphe mwana wake akhwimire.
koma munthu yemwe adatitsina khutu za nkhaniyi, adati bamboyo adakatenga mankhwala oti alemere ndipo adauzidwa kuti akwilire mankhwalawo mnyumba kuti aphe mwana wake akhwimire.
female
Atachita izi mwana wakeyo atalowa mnyumamo adakomoka koma mwachangu mkazi wake adakafukula mankhwalawo mwanayo nkusisika, ndipo pomwepo bamboyo adachita misala,adatero iwo.
Atachita izi mwana wakeyo atalowa mnyumamo adakomoka koma mwachangu mkazi wake adakafukula mankhwalawo mwanayo nkusisika, ndipo pomwepo bamboyo adachita misala,adatero iwo.
female
A Sipiriyano adatsimikiza zoti bamboyo adachita misala tsabata ziwiri zapitazo koma adakachira ku mapemphero kumabwerera kumudzi komwe atangofika adapha mkazi wakeyo
A Sipiriyano adatsimikiza zoti bamboyo adachita misala tsabata ziwiri zapitazo koma adakachira ku mapemphero kumabwerera kumudzi komwe atangofika adapha mkazi wakeyo
female
Lipoti lomwe talandira ndiloti atachira kubwerera kumudzi pa 10 october, anthu adadabwa atatenga ana ake awiri nkuloweranawo kwa agogo awo modabwitsa.
Lipoti lomwe talandira ndiloti atachira kubwerera kumudzi pa teni okotobala, anthu adadabwa atatenga ana ake awiri nkuloweranawo kwa agogo awo modabwitsa.
female
ndipo anthuwo atathamangira kunyumba kwake adakapeza mkazi wake atagona mmagazi. Adatero a Sipiriyano.
ndipo anthuwo atathamangira kunyumba kwake adakapeza mkazi wake atagona mmagazi. Adatero a Sipiriyano.
female
iwo ati bamboyo ndi malemu mkazi wakeyo, onse amachokera mmudzi mwa MtheKo kwa mfumu yayikulu Mwambo, mboma la Zomba.
iwo ati bamboyo ndi malemu mkazi wakeyo, onse amachokera mmudzi mwa MtheKo kwa mfumu yayikulu Mwambo, mboma la Zomba.
female
Nako ku Chiradzulu, banja lina lili mmanja mwa police, powaganizira kuti adapha mwana wawo wa miyezi 5 chifukwa bambo wa mnyumbamo a Robart Miliyasi azaka 27 amakaika kuti mwanayo ndiwawo.
Nako ku Chiradzulu, banja lina lili mmanja mwa polisi, powaganizira kuti adapha mwana wawo wa miyezi fayifi chifukwa bambo wa mnyumbamo a Robati Miliyasi azaka tuwente-seveni amakaika kuti mwanayo ndiwawo.
female
Mneneri wa police ya Chiradzulu a Cosmas Kagulo, ati banjalo lidayamba mchaka cha 2018 mkaziyo ali kale ndi ana awiri, ndipo akhala akulekana nkubwereranaso katatu konse.
Mneneri wa polisi ya Chiradzulu a Kosimasi Kagulo, ati banjalo lidayamba mchaka cha tuwente-eyitini mkaziyo ali kale ndi ana awiri, ndipo akhala akulekana nkubwereranaso katatu konse.
female
Iwo ati ulendo womaliza, mkaziyo Regina Thomas wazaka 22, adali ndi pakati koma bamboyo amkakayi kuti mimbayo idali yake.
Iwo ati ulendo womaliza, mkaziyo Rejina Thomasi wazaka tuwente-thu, adali ndi pakati koma bamboyo amkakayi kuti mimbayo idali yake.
female
mpakana adasiyananso mkaziyo nkubwelera kwawo. Kafukufuku wathu wapeza kuti mwana atabadwa mwezi wa may 2023,
mpakana adasiyananso mkaziyo nkubwelera kwawo. Kafukufuku wathu wapeza kuti mwana atabadwa mwezi wa meyi tuwente tuwente-firi,
female
Mayiyo adapereka maganizo oti angomupha kuti asasokoneza banjalo. Ndipo adayesa kawiri konse kuti aphe mwanayo koma zimavuta.
Mayiyo adapereka maganizo oti angomupha kuti asasokoneza banjalo. Ndipo adayesa kawiri konse kuti aphe mwanayo koma zimavuta.
female
pa 4 October, 2023, mkazi uja adazondotsera mwanayo mndowa yodzadza ndi madzi mpaka adafa, keneko adamubereka ngati ali moyo.
pa folo Okotobala, tuwente tuwente-firi, mkazi uja adazondotsera mwanayo mndowa yodzadza ndi madzi mpaka adafa, keneko adamubereka ngati ali moyo.
female
nkupitanaye kwa makolo ake komwe adazindikira kuti mwanyo ndi nchitanda, atero a Kagulo.
nkupitanaye kwa makolo ake komwe adazindikira kuti mwanyo ndi nchitanda, atero a Kagulo.
female
Iwo ati abalewo atapanikiza mayiyo ndi mwamuna wake adavomera kuti adapha manayo ndipo nkhani idanka kwa mfumu omwe adayipititsa ku police.
Iwo ati abalewo atapanikiza mayiyo ndi mwamuna wake adavomera kuti adapha manayo ndipo nkhani idanka kwa mfumu omwe adayipititsa ku polisi.
female
Pano banjalo lomwe limachokera mmudzi mwa Misomali kwa mfumu Mkalo, lili mmanja mwa police ndipo likuyembekezera kukayankha mulandu wakupha
Pano banjalo lomwe limachokera mmudzi mwa Misomali kwa mfumu Mkalo, lili mmanja mwa polisi ndipo likuyembekezera kukayankha mulandu wakupha
female
Ndipo ku Chitipa, mnyamata wa zaka 15 akumuganizira kuti adapha agogo wake powasinga khosi ndi chikwakwa powaganizira kuti adapha a bambo wake mmatsenga.
Ndipo ku Chitipa, mnyamata wa zaka fifitini akumuganizira kuti adapha agogo wake powasinga khosi ndi chikwakwa powaganizira kuti adapha a bambo wake mmatsenga.
Mneneri wa police ku Chitipa a Gladwel Simwaka atsimikiza, koma pomwe timalemba nkhaniyi nkuti asanatitumizire nkhani yonse momwe idakhalira kuti zifike poti mwanayo aphe agogowo
Mneneri wa polisi ku Chitipa a Giladiwelo Simwaka atsimikiza, koma pomwe timalemba nkhaniyi nkuti asanatitumizire nkhani yonse momwe idakhalira kuti zifike poti mwanayo aphe agogowo
female
Akadaulo pa nkhani zosiyanasiyana mdziko muno ati mbale yotsutsa boma ili ndi benthu lake pa mavuto omwe a Malawi akudutsamo chifukwa mbaliyo yalephera kugwira ntchito yake moyenera.
Akadaulo pa nkhani zosiyanasiyana mdziko muno ati mbale yotsutsa boma ili ndi benthu lake pa mavuto omwe a Malawi akudutsamo chifukwa mbaliyo yalephera kugwira ntchito yake moyenera.
female
malingana ndi kadaulo pa ndale a Enerst Thundwa, udindo wa otsutsa boma ndikuuniira pomwe boma likulephera ndi kupereka maganizo awo
malingana ndi kadaulo pa ndale a Enesiti Thundwa, udindo wa otsutsa boma ndikuuniira pomwe boma likulephera ndi kupereka maganizo awo
female
pa momwe zinthu zikuyenera kuyendera kuwonetsa momwe iwo angakonzere zithu atalowa m'boma
pa momwe zinthu zikuyenera kuyendera kuwonetsa momwe iwo angakonzere zithu atalowa m'boma
female
koma a Thindwa ati otsutsa alero akukhala ngati ali mtulo kapena akukhalira dala chete kuti adazepeze chonena nthawi yokopa anthu ya kampeni ikadzafika
koma a Thindwa ati otsutsa alero akukhala ngati ali mtulo kapena akukhalira dala chete kuti adazepeze chonena nthawi yokopa anthu ya kampeni ikadzafika
female
pomwe akuyembekezeka kudzagwiritsa ntchito kufooka kwa anzawo, otsutsatu ndi boma la chiyembekezo. Ndiye zimafunika kuwonetsa chiyembekezocho pomwe mukutsutsa, osati kudikira za agwetsa nditola ayi.

anthu akawona momwe mukuperekera mfundo ku boma la nthawi imeneyo, ndipomwe amakhala nanu ndi chiyembekezo, atero a Thindwa
anthu akawona momwe mukuperekera mfundo ku boma la nthawi imeneyo, ndipomwe amakhala nanu ndi chiyembekezo, atero a Thindwa
female
Pomwe kadaulo pazachuma a Christopher Mbukwa omwe amaphunzitsa ku school ya ukachenjede ya Mzuzu University, ati mbali yotsutsa ya ulendo uno ikungokhala ngati ili mbali ya boma.
Pomwe kadaulo pazachuma a khirisitofa Mbukwa omwe amaphunzitsa ku sukulu ya ukachenjede ya Mzuzu Univesite, ati mbali yotsutsa ya ulendo uno ikungokhala ngati ili mbali ya boma
female
chifukwa ikulekerera chilichonse chibwino ndi choipa chomwe. Iwo ati mwachitsanzo powona momwe ndondomeke ya zipangizo za uli zotsitsa mtengo ya AIP ikulephelera,
chifukwa ikulekerera chilichonse chibwino ndi choipa chomwe. Iwo ati mwachitsanzo powona momwe ndondomeke ya zipangizo za uli zotsitsa mtengo ya eayepi ikulephelera,
female
Otsutsa amayenera kukwera pachulu kulimbana ndi boma kuti pologalamuyi isinthidwe, koma nawo angotsatira mbuyo. Vuta lakula ndi ndale
Otsutsa amayenera kukwera pachulu kulimbana ndi boma kuti pologalamuyi isinthidwe, koma nawo angotsatira mbuyo. Vuta lakula ndi ndale.
female
Aliyense amatenga ngati pologaklamu ya eayepi ndiye chopambanira zisankho. Ndiye ngakhale ikulephera kuonetsa zipatso zoyenera, otsutsa sakuyankhulapoi kanthu, moti kuti ipite ku nyumba ya malamulo akayisapotanso
Aliyense amatenga ngati pologaklamu ya AIP ndiye chopambanira zisankho. Ndiye ngakhale ikulephera kuonetsa zipatso zoyenera, otsutsa sakuyankhulapoi kanthu, moti kuti ipite ku nyumba ya malamulo akayisapotanso
female