audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
A Chimwemwe Zololo, atha masiku 6 mchitokosi cha police ku Zomba, powaganizira kuti amafuna kugulitsa mwana wompeza
A Chimwemwe Zololo, atha masiku sikisi mchitokosi cha polisi ku Zomba, powaganizira kuti amafuna kugulitsa mwana wompeza
female
A Zololo, akuyembekezereka kukawonekera ku bwalo lamilandu, komwe akuyankha mlandu malinga ndi m’neneri wa police ku Zomba a Aaron Chilala.
A Zololo, akuyembekezereka kukawonekera ku bwalo lamilandu, komwe akuyankha mlandu malinga ndi m’neneri wa polisi ku Zomba a Aroni Chilala.
female
Iwo anati, nkhaniyi idachitika loweruka pa 27 January,2024, pamene a Zololo adayika pa msika mwanayo, ndicholinga choti achepetse mavuto azachuma pakhomo pawo.
Iwo anati, nkhaniyi idachitika loweruka pa tuwente seveni Januware, tuwente tuwente folo, pamene a Zololo adayika pa msika mwanayo, ndicholinga choti achepetse mavuto azachuma pakhomo pawo.
female
Mneneriyu anati amatsata mwanayo, yemwe ndi wazaka ziwiri mmudzi mwa Njala.Kumeneku akuti kunali wamalonda amene adadyerera maso pa malondawo.
Mneneriyu anati amatsata mwanayo, yemwe ndi wazaka ziwiri mmudzi mwa Njala.Kumeneku akuti kunali wamalonda amene adadyerera maso pa malondawo.
female
A Chilala anapitiriza kunena kuti a Zololo ndi wa business yu, adagwirizana kuti akakumane mmudzimo nthawi ya 4 koloko madzulo, kuti akamvane za mtengo.
A Chilala anapitiriza kunena kuti a Zololo ndi wa bizinesiyu, adagwirizana kuti akakumane mmudzimo nthawi ya folo koloko madzulo, kuti akamvane za mtengo.
female
Koma a Zololo samadziwa kuti wamalondayu, wawamenya m’mimba kambakoti adatsina khutu a police kuti adzadziwonere wokha.
Koma a Zololo samadziwa kuti wamalondayu, wawamenya m’mimba kambakoti adatsina khutu a polisi kuti adzadziwonere wokha.
female
Tidafika pamalopo, ndipo timamva awiriwo akukambirana za mtengo, sitidachedwe komwe kuwambwandira a Zololo adatero Chilala.
Tidafika pamalopo, ndipo timamva awiriwo akukambirana za mtengo, sitidachedwe komwe kuwambwandira a Zololo adatero Chilala.
female
Iwo adati atafika ku police adayimbira phone akazi awo, kuti adzave zomwe amuna awo achita.
Iwo adati atafika ku polisi adayimbira phone akazi awo, kuti adzave zomwe amuna awo achita.
female
A police adagwira pakamwa, mkaziyo akunena mmaso muli gwaa! Kuti nkhaniyo idayamba kukambidwa kunyumba kwawo, kuti aphetse mwanayo.
A polisi adagwira pakamwa, mkaziyo akunena mmaso muli gwaa! Kuti nkhaniyo idayamba kukambidwa kunyumba kwawo, kuti aphetse mwanayo.
female
Koma mkaziyo adatiuza kuti ganizo lofuna kugulitsa mwana lidachokera kwa mwamunayo, ndipo mkaziyo adakana kuti zimenezo zisachitike.
Koma mkaziyo adatiuza kuti ganizo lofuna kugulitsa mwana lidachokera kwa mwamunayo, ndipo mkaziyo adakana kuti zimenezo zisachitike.
female
Mkaziyo adati, chifukwa chogulitsira mwanayo, kudalikuti akonze mavuto azachuma amena ali m’banja lawo, adatero a Chilala.
Mkaziyo adati, chifukwa chogulitsira mwanayo, kudalikuti akonze mavuto azachuma amena ali m’banja lawo, adatero a Chilala.
female
Lachinayi a Zololo adakawonekera kubwalo la milandu ku Zomba, komwe adaukana mulanduwo. A court, awuyimitsa kaye mpaka pa 8 February,2024.
Lachinayi a Zololo adakawonekera kubwalo la milandu ku Zomba, komwe adaukana mulanduwo. A khoti, awuyimitsa kaye mpaka pa eyiti Febuluwale, tuwente tuwente folo.
female
Bambowa omwe ali ndi zaka 25, amachokera m’mudzi mwa Chimbalanga kwa mfumu Chiwalo, m’boma la Phalombe.
Bambowa omwe ali ndi zaka tuwente faifi, amachokera m’mudzi mwa Chimbalanga kwa mfumu Chiwalo, m’boma la Phalombe.
female
Mwana wa zaka 15, ali m’manja mwa a police ku Mangochi, pomuganizira kuti adazimitsa mchemwali wake, wa zaka 26, pa mkangano wa poto, woti akazingire chimanga.
Mwana wa zaka fifitini, ali m’manja mwa a polisi ku Mangochi, pomuganizira kuti adazimitsa mchemwali wake, wa zaka tuwente sikisi, pa mkangano wa poto, woti akazingire chimanga.
female
Malinga ndi m’neneri wa police m’bomali Amina Tepani Daudi, mwanayo akuti njala itamupola, adaganiza zokazinga chimanga kuti mwina angayike kanthu m’mimba.
Malinga ndi m’neneri wa polisi m’bomali Amina Tepani Dawudi, mwanayo akuti njala itamupola, adaganiza zokazinga chimanga kuti mwina angayike kanthu m’mimba.
female
Kukazinga chimanga sidali nkhani yolemetsa kwa chemwali akewo, koma pamene padakhota ndi poto amene mwanayo amagwiritsa ntchito.
Kukazinga chimanga sidali nkhani yolemetsa kwa chemwali akewo, koma pamene padakhota ndi poto amene mwanayo amagwiritsa ntchito.
female
Mwanayo akuti amakazingira chimanga mpoto wa nyuwani, amene mchemwaliyo amene lero ndi malemu adagula kumene, zomwe zidamuyabwa.
Mwanayo akuti amakazingira chimanga mpoto wa nyuwani, amene mchemwaliyo amene lero ndi malemu adagula kumene, zomwe zidamuyabwa.
female
Komabe kwa mwanayo akuti sadawone vuto, posinthana Chichewa, awiriwo akuti adagwirana mthupi.
Komabe kwa mwanayo akuti sadawone vuto, posinthana Chichewa, awiriwo akuti adagwirana mthupi.
female
Apa ndipamene mwanayo anaganiza zothawa, ndipo takhala tikumusaka koma sitimamupeza.
Apa ndipamene mwanayo anaganiza zothawa, ndipo takhala tikumusaka koma sitimamupeza.
female
Tidafalitsa uthenga kwa anthu komaso ofuna kwabwino, kuti atithandize kusaka mwanayo, adatero Daudi.
Tidafalitsa uthenga kwa anthu komaso ofuna kwabwino, kuti atithandize kusaka mwanayo, adatero Daudi.
female
Iye adati, mayi wa anawo, adathamanga ndi mtsikanayo ku chipatala kuti akalandire thandizo, koma a chipatala adasowa pogwira chifukwa nkuti atamwalira kale.
Iye adati, mayi wa anawo, adathamanga ndi mtsikanayo ku chipatala kuti akalandire thandizo, koma a chipatala adasowa pogwira chifukwa nkuti atamwalira kale.
female
Zotsatira za chipatala zidapeza kuti mtsikanayo adatisiya chifukwa adataya magazi ambiri, adatero Daudi.
Zotsatira za chipatala zidapeza kuti mtsikanayo adatisiya chifukwa adataya magazi ambiri, adatero Daudi.
female
Apolice akhala akusaka woganiziridwayo, ndipo amunjata atamupeza m’boma la Balaka komwe ati amabisala pa malo ena ogulitsa mowa.
Apolisi akhala akusaka woganiziridwayo, ndipo amunjata atamupeza m’boma la Balaka komwe ati amabisala pa malo ena ogulitsa mowa.
female
Tidatsinidwa khutu ndi ofuna kwabwino omwe adati mwanayo akuwoneka ku Balaka ndipo tidadziwitsa a police ya Balaka, amene amunjata, adamupeza pamalo omwera mowa a Mgawanyemba, adatero.
Tidatsinidwa khutu ndi ofuna kwabwino omwe adati mwanayo akuwoneka ku Balaka ndipo tidadziwitsa a polisi ya Balaka, amene amunjata, adamupeza pamalo omwera mowa a Mgawanyemba, adatero.
female
Mkazi wa Inkosi ya Makosi Gomani 5 Inkosikati Lichaladza Khanyisa Gomani.
Mkazi wa Inkosi ya Makosi Gomani faifi Inkosikati Lichaladza Khanyisa Gomani.
female
Wati kuchuluka kwa mimba za ana a chichepere, kukukolezera kusachita bwino kwa ana a school pa meyeso a MANEB, m’bomali.
Wati kuchuluka kwa mimba za ana a chichepere, kukukolezera kusachita bwino kwa ana a sukulu pa meyeso a MANEBU, m’bomali.
female
A Gomani adanena izi, pomwe adatsagana ndi mlangizi wa boma pa nkhani za uchembere wabwino, mayi Dorothy Ngoma, kukayendera mayi wina wa zaka 29.
A Gomani adanena izi, pomwe adatsagana ndi mlangizi wa boma pa nkhani za uchembere wabwino, mayi Dorofe Ngoma, kukayendera mayi wina wa zaka tuwente nayini.
female
Ledina Paul, yemwe anabereka ana asanu, pa chipatala cha m’boma la Ntcheu. Iwo anati mwachitsanzo zotsatira za mayeso a boma zaka zapitazi
Ledina Poo, yemwe anabereka ana asanu, pa chipatala cha m’boma la Ntcheu. Iwo anati mwachitsanzo zotsatira za mayeso a boma zaka zapitazi
female
Boma la Ntcheu, lakhala likupezeka ku mapeto kwenikweni, kwa maboma omwe sanachitebwino pa mayesowa.
Boma la Ntcheu, lakhala likupezeka ku mapeto kwenikweni, kwa maboma omwe sanachitebwino pa mayesowa.
female
Mimba zomwe atsikana akumatenga zikukolezera kwambiri m’chitidwe wosiyira sukulu pa njira, popeza atsikanawa tsopano akumayika chidwi chawo posamala makanda.
Mimba zomwe atsikana akumatenga zikukolezera kwambiri m’chitidwe wosiyira sukulu pa njira, popeza atsikanawa tsopano akumayika chidwi chawo posamala makanda.
female
Omwe abereka, zomwe zikumasokonezaso ngakhale zotsatira za mayeso zikatula. Anadandaula motero.
Omwe abereka, zomwe zikumasokonezaso ngakhale zotsatira za mayeso zikatula. Anadandaula motero.
female
Iwo adapempha atsikana omwe anasiyira school pa njira Kamba ka uchembere, kuti abwerere kukayambaso school, komaso nkuwalimbikitsa kugwiritsa ntchito njira za kulera.
Iwo adapempha atsikana omwe anasiyira sukulu pa njira Kamba ka uchembere, kuti abwerere kukayambaso sukulu, komaso nkuwalimbikitsa kugwiritsa ntchito njira za kulera.
female
Kufikira pomwe adzafike podziyimira pawokha, ndiso kukhala ndi banja lokhazikika.
Kufikira pomwe adzafike podziyimira pawokha, ndiso kukhala ndi banja lokhazikika.
female
Ndipo mulangizi wa boma pa nkhani za uchembere wabwino, mayi Ngoma, adati ndi wokhudzika kwambiri, Kamba ka kuchuluka kwa atsikana omwe chiwerengero chawo chikukwera m’zipatala m’dziko muno.
Ndipo mulangizi wa boma pa nkhani za uchembere wabwino, mayi Ngoma, adati ndi wokhudzika kwambiri, Kamba ka kuchuluka kwa atsikana omwe chiwerengero chawo chikukwera m’zipatala m’dziko muno.
female
Ndizovetsa chisoni kuti ana a zaka 12, akupezeka m’zipinda zoberekeramo, komwe sakuyenera kupezeka. Izi zikudzetsa kuchulukana m’zipindazi, sitili wokozeka ngati dziko,
Ndizovetsa chisoni kuti ana a zaka twelofu, akupezeka m’zipinda zoberekeramo, komwe sakuyenera kupezeka. Izi zikudzetsa kuchulukana m’zipindazi, sitili wokozeka ngati dziko,
female
Kukhala ndi ana ochuluka chonchi m’zipatalamo chifukwa tikupatsa ntchito yayikulu kwambiri kwa azathu omwe amagwira ntchito m’zipatalamo. Adatero iwo.
Kukhala ndi ana ochuluka chonchi m’zipatalamo chifukwa tikupatsa ntchito yayikulu kwambiri kwa azathu omwe amagwira ntchito m’zipatalamo. Adatero iwo.
female
A Ngoma adalangiza achinyamata kuti apewe mchitidwe wogonana ali a chichepere ndipokuti m’malo mwake ayike chidwi kwambiri pa maphunziro kuti adzkhale nzika zodalirika.
A Ngoma adalangiza achinyamata kuti apewe mchitidwe wogonana ali a chichepere ndipokuti m’malo mwake ayike chidwi kwambiri pa maphunziro kuti adzkhale nzika zodalirika.
female
Mwachitsanzo, amayi achicheperewa, akuwapeza m’zipatalamu atabereka, amachita kuwoneka kuti alibe zoyenereza kulera anawa kumbali yachuma komaso thandizo lina.
Mwachitsanzo, amayi achicheperewa, akuwapeza m’zipatalamu atabereka, amachita kuwoneka kuti alibe zoyenereza kulera anawa kumbali yachuma komaso thandizo lina.
female
Izi zikuthandiza kukolezeraso umphawi m’dzikomuno, adaonjeza motero.
Izi zikuthandiza kukolezeraso umphawi m’dzikomuno, adaonjeza motero.
female
Mkulu wa anamwino pa chipatala cha Ntcheu, mayi Gloria Magombo, adavomereza zoti mzipatala za m’bomalo akulandira ana ochuluka omwe amapita ukachira m’zipatalazi.
Mkulu wa anamwino pa chipatala cha Ntcheu, mayi Guloriya Magombo, adavomereza zoti mzipatala za m’bomalo akulandira ana ochuluka omwe amapita ukachira m’zipatalazi.
female
Zomwe ati iliso lakhala vuto lalikulu, poti atsikana achichepere amakhala pa ziopsyezo zazikulu pobereka. Tikukhaladi ndi chiwerengero chochuluka cha amayi omwe akumabwera kudzabereka.
Zomwe ati iliso lakhala vuto lalikulu, poti atsikana achichepere amakhala pa ziopsyezo zazikulu pobereka. Tikukhaladi ndi chiwerengero chochuluka cha amayi omwe akumabwera kudzabereka.
female
Ena mwaiwo ndi achichepere, motipatsiku timachiza amayi oposa 24, koma nthawizina pachipatala pokhapano, timathaso kubadwitsa ana mpaka 30 pa tsiku limodzi, adatero iwo.
Ena mwaiwo ndi achichepere, motipatsiku timachiza amayi oposa tuwente folo, koma nthawizina pachipatala pokhapano, timathaso kubadwitsa ana mpaka sete pa tsiku limodzi, adatero iwo.
female
Chaka cha 2023, chikupita ndi nkhani zake, imodzi mwa nkhani zimene zidayala nthenje ndiyamsungwana wa zaka 14.
Chaka cha tuwente tuwente-fifi, chikupita ndi nkhani zake, imodzi mwa nkhani zimene zidayala nthenje ndiyamsungwana wa zaka fotini.
female
Yemwe amayimba school mu standard 5, atakamang’ala ku court kuti limasulirebwino, zifukwa zomwe amayi angaloledwe kuchotsa pakati.
Yemwe amayimba sukulu mu sitandade faifi, atakamang’ala ku khoti kuti limasulirebwino, zifukwa zomwe amayi angaloledwe kuchotsa pakati.
female
Izi zidadza pomwe mabungwe ena akumenyera kuti lamulo lochotsa mimba, lisinthidwe mogwirizana ndizimene idapeza commission yosakatula malamulo adziko lino ya Law commission.
Izi zidadza pomwe mabungwe ena akumenyera kuti lamulo lochotsa mimba, lisinthidwe mogwirizana ndizimene idapeza komishoni yosakatula malamulo adziko lino ya Lo komishoni.
female
Bungwero lidati lamulolo lisinthidwe, kuti awonjezere zifukwa zimene amayi angachotsere mimba, kupatula zoti kuchotsa mimbako kuchitike ngati ingayike pa chiopsyezo umoyo wa amayi.
Bungwero lidati lamulolo lisinthidwe, kuti awonjezere zifukwa zimene amayi angachotsere mimba, kupatula zoti kuchotsa mimbako kuchitike ngati ingayike pa chiopsyezo umoyo wa amayi.
female
Iyo idati lamulolo liwonjezere kuti amayi angachotse mimba, ngati mayi anapatsidwa mimba atagwiriridwa kapena kupatsidwa ndi m’balewake.
Iyo idati lamulolo liwonjezere kuti amayi angachotse mimba, ngati mayi anapatsidwa mimba atagwiriridwa kapena kupatsidwa ndi m’balewake.
female
Msungwana adakamang’alayo, adagwiriridwa ndi njonda ina yomwe pano ikuseweza zaka 14 kundende koma akuti atapita ku chipatala.
Msungwana adakamang’alayo, adagwiriridwa ndi njonda ina yomwe pano ikuseweza zaka fotini kundende koma akuti atapita ku chipatala.
female
Kuti amuthandize kuchotsa mimba yomwe idabwera Kamba kogwiriridwako, koma kuchipatala adakana pemphoro.
Kuti amuthandize kuchotsa mimba yomwe idabwera Kamba kogwiriridwako, koma kuchipatala adakana pemphoro.
female
Malingana ndi kafukufuku, yemwe adachita akadawulo ku school ya ukachenjede wa zaumoyo ya Kamuzu University of Health Sciencies (KUHESI).
Malingana ndi kafukufuku, yemwe adachita akadawulo ku sukulu ya ukachenjede wa zaumoyo ya Kamuzu Univesite of Hefe Sayansezi (KUHESI).
female
Okhudza asungwana omwe sadafike zaka 18, ndipo adatenga mimba Kamba kogwiriridwa, moyo wawo umakhala pa chiopsyezo.
Okhudza asungwana omwe sadafike zaka eyitini, ndipo adatenga mimba Kamba kogwiriridwa, moyo wawo umakhala pa chiopsyezo.
female
Ambiri mwa asungwana omwe adatenga mbali pa kafukufukuyu, adati amaonangati moyo wawo wasokonekera monga.
Ambiri mwa asungwana omwe adatenga mbali pa kafukufukuyu, adati amaonangati moyo wawo wasokonekera monga.
female
Moti amalingalira zongozipha poona kuti tsogolo lawo lawonongeka. Zikutero zotsatira za kafukufukuyo.
Moti amalingalira zongozipha poona kuti tsogolo lawo lawonongeka. Zikutero zotsatira za kafukufukuyo.
female
Mabungwe a Centre for Human Rights and Rehalbilitation, CHRR, Nyali Institute, Young Women Consortium, Centre for Reproductive Rights.
Mabungwe a senata for Humani Rayitsi and Rehabiliteshoni (CHRR), Nyali Insitichuti, Yang'i Wimeni's konzotiyamu, senta fo Repurodakitivi Rayitsi.
female
Ndi ya Afia Nahak, ati athandiza msungwanayo mpaka pomwe court lidzagamule nkhaniyake.
Ndi ya Afiya Nahaki, ati athandiza msungwanayo mpaka pomwe khoti lidzagamule nkhaniyake.
female
Mkulu wa bungwe la CHRR, a Michael Kayiyatsa, ati nkhaniyi sikukhudza m’tsutso omwe ulipokale woti malamulo adzirola atsikana ndi asungwana kuchotsa mimba ngati afuna kutero.
Mkulu wa bungwe la si etchi ara ara, a Mayikolo Kayiyatsa, ati nkhaniyi sikukhudza m’tsutso omwe ulipokale woti malamulo adzirola atsikana ndi asungwana kuchotsa mimba ngati afuna kutero.
female
Tikudziwa kuti palikale m’tsutso okhudza kuchotsa mimba, nkhani ya msungwanayu sikukhudza m’tsutso umenewo ayi.
Tikudziwa kuti palikale m’tsutso okhudza kuchotsa mimba, nkhani ya msungwanayu sikukhudza m’tsutso umenewo ayi.
female
Apa mwanayu, akungofuna court limasulire ngati angathe kuchotsa mimba yakeyo. Atero a Kayiyatsa.
Apa mwanayu, akungofuna khoti limasulire ngati angathe kuchotsa mimba yakeyo. Atero a Kayiyatsa.
female
Yemwe akuyendetsa nkhaniyo ku bungwe la CHRR, a Dennis Mwafulirwa, adati mkulu yemwe adagwiririra msungwanayu, adagwidwa ndipo akuseweza zaka 14.
Yemwe akuyendetsa nkhaniyo ku bungwe la si etchi ara ara, a Denisi Mwafulirwa, adati mkulu yemwe adagwiririra msungwanayu, adagwidwa ndipo akuseweza zaka fotini.
female
Koma adati, pali chiletso cha court, choti zambiri za msungwanayu zisawululidwe, pali nkhani ya chitetezo cha msungwanayo, monga mudziwa kuti ndi mwana wa mng’ono, ndiye a court aletsa kuwulula zina ndi zina.
Koma adati, pali chiletso cha khoti, choti zambiri za msungwanayu zisawululidwe, pali nkhani ya chitetezo cha msungwanayo, monga mudziwa kuti ndi mwana wa mng’ono, ndiye a khoti aletsa kuwulula zina ndi zina.
female
Chomwe tikuopa kwambiri nchoti ena akava za komwe amachokera kaya mbiri ya school, akhoza kumufufuza mpaka kumupeza. Atero a Mwafulirwa.
Chomwe tikuopa kwambiri nchoti ena akava za komwe amachokera kaya mbiri ya sukulu, akhoza kumufufuza mpaka kumupeza. Atero a Mwafulirwa.
female
Koma iwo ati, nkhaniyo itangochitika, Office yowona za chisamaliro cha ana, idatenga mtsikanayo, ndikukamusungitsa ku nyumba ya chitetezo.
Koma iwo ati, nkhaniyo itangochitika, Ofesi yowona za chisamaliro cha ana, idatenga mtsikanayo, ndikukamusungitsa ku nyumba ya chitetezo.
female
Chifukwa cha chitozo chomwe amalandira m’mudzimo, komaso yemwe adamupanga chipongweyo, amakhala m’mudzi momwemo.
Chifukwa cha chitozo chomwe amalandira m’mudzimo, komaso yemwe adamupanga chipongweyo, amakhala m’mudzi momwemo.
female
Chikalata chomwe mabungwewo adatulutsa limodzi, chikuti mimba zobwera Kamba kogwiriridwa, zimakhala ndi ziopsyezo zambiri pa moyo wa ogwiriridwayo.
Chikalata chomwe mabungwewo adatulutsa limodzi, chikuti mimba zobwera Kamba kogwiriridwa, zimakhala ndi ziopsyezo zambiri pa moyo wa ogwiriridwayo.
female
Munthu akagwirirdwa, chiopsyezo choyamba nkusalidwa m’mudzi, komaso poti ena amakhala a chichepere, moyo wawo umakhala pa ciopsyezo.
Munthu akagwirirdwa, chiopsyezo choyamba nkusalidwa m’mudzi, komaso poti ena amakhala a chichepere, moyo wawo umakhala pa ciopsyezo.
female
Ena monga mwavakale amakhala ndi malingaliro odzipha, chatero chikalatacho. Mabugwewo ati kuwunikira kwa court pa nkhani ya msungwanayo.
Ena monga mwavakale amakhala ndi malingaliro odzipha, chatero chikalatacho. Mabugwewo ati kuwunikira kwa khoti pa nkhani ya msungwanayo.
female
Kukhoza kutsegula khomo la ufulu wa amsungwana ambiri omwe amatenga mimba Kamba kogwiriridwa, koma amakakamizidwa kusunga mimbayo poopa malamulo.
Kukhoza kutsegula khomo la ufulu wa amsungwana ambiri omwe amatenga mimba Kamba kogwiriridwa, koma amakakamizidwa kusunga mimbayo poopa malamulo.
female
Nduna ya zachitetezo cha m’dziko a Ken Zikhale Ng’oma ati unduna wawo wakhwimitsa chitetezo, mnyengo ya zisangalalo za Christmass ndi nyuwere, kuti a Malawi asangalale mwa ufulu
Nduna ya zachitetezo cha m’dziko a Keni Zikhale Ng’oma ati unduna wawo wakhwimitsa chitetezo, mnyengo ya zisangalalo za Khirisimasi ndi nyuwere, kuti a Malawi asangalale mwa ufulu
female
Koma akadaulo pa zachuma a Millward Tobias, achenjeza kuti poyandikira chisangalalochi, makolo asayiwale kuti mwezi wa January 2024, afunika kupereka ma fees, komaso kuyendetsa za kumunda.
Koma akadaulo pa zachuma a Miliwadi Tobiyasi, achenjeza kuti poyandikira chisangalalochi, makolo asayiwale kuti mwezi wa Januware tuwente tuwente folo, afunika kupereka ma fizi, komaso kuyendetsa za kumunda.
female
Iwo anena izi, potengera momwe chuma chikuyendera m’dzikomuno, potsatira kugwa kwa ndalama ya kwacha, komwe kwakweza mitengo ya zinthu.
Iwo anena izi, potengera momwe chuma chikuyendera m’dzikomuno, potsatira kugwa kwa ndalama ya kwacha, komwe kwakweza mitengo ya zinthu.
female
Dziko lapansi makamaka a Khristu, akhala akukondwerera christmass ndi chaka chatsopano, nyuwere kuyamba pa 24 December 2023 mpaka pa 02 January,2024.
Dziko lapansi makamaka a Khirisitu, akhala akukondwerera khirisimasi ndi chaka chatsopano, nyuwere kuyamba pa tuwente folo Disembala tuwente tuwenye firi mpaka pa thu Januware, tuwente tuwente folo.
female
Panyengoyi, kumakhala maphwando komaso kugula zovala ndi mphatso zosiyanasiyana, zomwe zimatenga ndalama zochuluka, makamaka potengeraso kuti anthu amalandira malipiro awo mnsanga.
Panyengoyi, kumakhala maphwando komaso kugula zovala ndi mphatso zosiyanasiyana, zomwe zimatenga ndalama zochuluka, makamaka potengeraso kuti anthu amalandira malipiro awo mnsanga.
female
A Tobias, omweso akufuna kudzayimira pa mpando wa president m’chaka cha 2025, ati zisangalalo ngati izi, zimapangitsa kuti pofika mwenzi wa January, anthu ambiri akhale alibe ndalama.
A Tobiyasi, omweso akufuna kudzayimira pa mpando wa purezidenti m’chaka cha tuwente tuwente fayifi, ati zisangalalo ngati izi, zimapangitsa kuti pofika mwenzi wa Januware, anthu ambiri akhale alibe ndalama.
female
Zimakhala zomvetsa chisoni, kuona makolo akusowa pogwira, ena mpaka ana kumadikira kuti alandire malipiro a January, kuti apite ku school. Uku nkulephera kokonzekera kwa kholo. Atero a Tobias.
Zimakhala zomvetsa chisoni, kuona makolo akusowa pogwira, ena mpaka ana kumadikira kuti alandire malipiro a Januware, kuti apite ku sukulu. Uku nkulephera kokonzekera kwa kholo. Atero a Tobiyasi.
female
Iwo ati, makolo anzeru, amayenera kuyika padera ndalama za fees ndi kumunda, nkuona kuti zotsalazo angapangenazo bwanji kuti banja lisangalale, uku akudziwa chichita mu January.
Iwo ati, makolo anzeru, amayenera kuyika padera ndalama za fizi ndi kumunda, nkuona kuti zotsalazo angapangenazo bwanji kuti banja lisangalale, uku akudziwa chichita mu Januware.
female
A Zikhale Ng’oma ati, a Malawi akamapanga ma programme awo azisangalalo, azipanga mtima uli m’malo kuti chitetezo ali nacho kuchokera ku unduna wawo.
A Zikhale Ng’oma ati, a Malawi akamapanga ma pulogaramu awo azisangalalo, azipanga mtima uli m’malo kuti chitetezo ali nacho kuchokera ku unduna wawo.
female
Ndimanena nthawi zambiri kuti boma ili, liri ndichidwi pankhani ya chitetezo, pano ndikutsimikizira a Malawi.
Ndimanena nthawi zambiri kuti boma ili, liri ndichidwi pankhani ya chitetezo, pano ndikutsimikizira a Malawi.
female
Kuti tiwapatsa chitetezo chokwanira mu nyengo ya zisangalalo ndipo yemwe akufuna kuyesa chitetezochi, ayese. Atero a Ng’oma.
Kuti tiwapatsa chitetezo chokwanira mu nyengo ya zisangalalo ndipo yemwe akufuna kuyesa chitetezochi, ayese. Atero a Ng’oma.
female
Nyengo ngati iyi, umbava, Umbanda ndi ngozi za mitundu yosiyanasiyana zimachuluka, koma a Ng’oma ati, unduna wawo, wakhazikitsa ndondomeko zokhwima.
Nyengo ngati iyi, umbava, Umbanda ndi ngozi za mitundu yosiyanasiyana zimachuluka, koma a Ng’oma ati, unduna wawo, wakhazikitsa ndondomeko zokhwima.
female
AMalawi sasadabwe akaona a police ali balalabalala m’madera mwawo, sikuti akukawamanga ayi. Koma ndi njira imodzi yomwe takhazikitsa, kuti paliponse pazipezeka a police.
AMalawi sasadabwe akaona a polisi ali balalabalala m’madera mwawo, sikuti akukawamanga ayi. Koma ndi njira imodzi yomwe takhazikitsa, kuti paliponse pazipezeka a polisi.
female
Kupatula apo, muona zipata za chipikisheni, zongokhazikitsa mwadzidzidzi m’misewumu.
Kupatula apo, muona zipata za chipikisheni, zongokhazikitsa mwadzidzidzi m’misewumu.
female
A police anjinga zamoto, magalimoto ndi oyenda pansi, akhala paliponse m’madera azisangalalo, kuti ateteze anthu. Atero a Ng’oma.
A polisi anjinga zamoto, magalimoto ndi oyenda pansi, akhala paliponse m’madera azisangalalo, kuti ateteze anthu. Atero a Ng’oma.
female
Undunawo atinso, kupatula kudalira apolice, chitetezo chachikulu cha munthu chimakhala ndi mwini wakeyo, moti anthu akuyenera kutsina khutu a police mnsanga akadabwa ndi zochita zawina.
Undunawo atinso, kupatula kudalira apolisi, chitetezo chachikulu cha munthu chimakhala ndi mwini wakeyo, moti anthu akuyenera kutsina khutu a polisi mnsanga akadabwa ndi zochita zawina.
female
Atinso oyendetsa galimoto, akuyenera kuwonetsetsa kuti galimoto zawo nzoyenera kuyendetsa pa mnseu, atsatire malamulo apa mnseu.
Atinso oyendetsa galimoto, akuyenera kuwonetsetsa kuti galimoto zawo nzoyenera kuyendetsa pa mnseu, atsatire malamulo apa mnseu.
female
Komaso omwe akuchoka pakhomo kukasangalala kwina akhwimitse chitetezo pakhomo pawo.
Komaso omwe akuchoka pakhomo kukasangalala kwina akhwimitse chitetezo pakhomo pawo.
female
Iwo adati, monga zakazonse, akunenaso kuti pochoka pakhomo, anthu asasiye popanda munthu ayi, osalengeza m’masamba a mchezo kuti simuli pakhomo.
Iwo adati, monga zakazonse, akunenaso kuti pochoka pakhomo, anthu asasiye popanda munthu ayi, osalengeza m’masamba a mchezo kuti simuli pakhomo.
female
Malinga ndi akulikulu la police ku Lilongwe, pakati pa 24 December, 2022 ndi 02 January, 2023. Anthu 20 adamwalira pomwe ena 70 adavulala pa ngozi.
Malinga ndi akulikulu la polisi ku Lilongwe, pakati pa tuwente folo Disembala, tuwente tuwente thu ndi thu Januware,c. Anthu tuwente adamwalira pomwe ena sevente adavulala pa ngozi
female
56 zomwe zidachitika panyengoyi. Pokonzekera chitetezochi, apolice m’maboma ena, ayamba kale kusesa anthu ophwanya malamulo.
56 zomwe zidachitika panyengoyi. Pokonzekera chitetezochi, apolisi m’maboma ena, ayamba kale kusesa anthu ophwanya malamulo.
female
Kuti panyengo ya zisangalalo, anthu otero, asasokoneze azawo, m’boma la Balaka, anthu 15 adagwidwa pachipikisheni cha pa 17 December,2018.
Kuti panyengo ya zisangalalo, anthu otero, asasokoneze azawo, m’boma la Balaka, anthu fifitini adagwidwa pachipikisheni cha pa zeventini Disembala, tuwente eyitini.
female
Pamilandu yosiyanasiyana monga, kuthyola ndi kuba, kupezeka nkatundu obedwa, kugonana ndi ana, kuvulaza azawo ndi kupezeka malo osayenera kupezekapo nthawi yolakwika.
Pamilandu yosiyanasiyana monga, kuthyola ndi kuba, kupezeka nkatundu obedwa, kugonana ndi ana, kuvulaza azawo ndi kupezeka malo osayenera kupezekapo nthawi yolakwika.
female
Mneneri wa police ya Mponera, a Mc Patson Msadala, ati kumenekonso apolice akhala akukumana ndi mafumu, anthu a m’midzi, ochita malonda ndi adindo ena, kukambirana nawo za chitetezo.
Mneneri wa polisi ya Mponera, a Maki Patisoni Msadala, ati kumenekonso apolisi akhala akukumana ndi mafumu, anthu a m’midzi, ochita malonda ndi adindo ena, kukambirana nawo za chitetezo.
female
A police amanga anthu 6, omwe akuwaganizira kuti adatengera lamulo m’manja mwawo, potengapo gawo pakuphedwa kwa abambo 4, omwe amaganiziridwa kuti amakaba m’boma la Thyolo.
A polisi amanga anthu sikisi omwe akuwaganizira kuti adatengera lamulo m’manja mwawo, potengapo gawo pakuphedwa kwa abambo folo omwe amaganiziridwa kuti amakaba m’boma la Thyolo.
female
Wachiwiri kwa m’neneri wa police m’dzikomuno a Alfred Chimthere, ati anthuwo amangidwa potsatira kafukufuku wa police.
Wachiwiri kwa m’neneri wa polisi m’dzikomuno a Alafuredi Chimthere, ati anthuwo amangidwa potsatira kafukufuku wa polisi.
female
Atalandira report loti abambo 4, adaphedwa pa 19, December 2023, kwa Njema mfumu yayikulu Mabuka, ku Thyolo.
Atalandira lipoti loti abambo folo, adaphedwa pa nayintini, Disembala tuwente tuwente firi, kwa Njema mfumu yayikulu Mabuka, ku Thyolo.
female
Anthuwa tawamanga chifukwa adaphwanya lamulo, timanena nthawi zambiri, kuti tikagwira munthu oganiziridwa mlandu, tizipitanaye ku police chifukwa amakhala akuthandiza pa kafukufuku. Atero a Chimthere.
Anthuwa tawamanga chifukwa adaphwanya lamulo, timanena nthawi zambiri, kuti tikagwira munthu oganiziridwa mlandu, tizipitanaye ku polisi chifukwa amakhala akuthandiza pa kafukufuku. Atero a Chimthere.
female
Iwo ati, kupatula kuphwanya lamulo, kupha woganiziridwa mlandu, ndikuphwanya ufulu wamunthu wokhala ndi moyo, komaso zimanyozetsa ulemu wamunthu wachilengedwe.
Iwo ati, kupatula kuphwanya lamulo, kupha woganiziridwa mlandu, ndikuphwanya ufulu wamunthu wokhala ndi moyo, komaso zimanyozetsa ulemu wamunthu wachilengedwe.
female
Nkhaniyi ikuti abamabo 4, adapezeka akukaba ku grocery ya wabusiness wina ku miseu 4, m’mudzi wa Njema kwa mfumu yayikulu Mabuka ku Thyolo.
Nkhaniyi ikuti abamabo folo, adapezeka akukaba ku golosale ya wabizinesi wina ku misewu folo, m’mudzi wa Njema kwa mfumu yayikulu Mabuka ku Thyolo.
female
Ndipo awiri adagwidwa, pomwe ena awiri adathawa. Nkhaniyo ikupitiriraso kuti awiri omwe adagwidwawo, adawulula azawo asadaphedwe.
Ndipo awiri adagwidwa, pomwe ena awiri adathawa. Nkhaniyo ikupitiriraso kuti awiri omwe adagwidwawo, adawulula azawo asadaphedwe.
female
Ndipo kenako anthuwo, adanka nasaka awiri enawo, omwe adawagwira adawaphaso.
Ndipo kenako anthuwo, adanka nasaka awiri enawo, omwe adawagwira adawaphaso.
female
Abambo omwe adaphedwawo, onse amachokera m’mudzi mwa Chipwayira, mfumu yayikulu Chikumbu, koyandikana ndi komwe amawaganizira kuti amafuna kubako.
Abambo omwe adaphedwawo, onse amachokera m’mudzi mwa Chipwayira, mfumu yayikulu Chikumbu, koyandikana ndi komwe amawaganizira kuti amafuna kubako.
female