audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Atero a Mbukwa. Iwo ati otsutsa amayenera kukhala pansi ndikusanthula vuto lililonse palokha ndikupeza mayankho ake ndi momwe mavutowo angathere.
Atero a Mbukwa. Iwo ati otsutsa amayenera kukhala pansi ndikusanthula vuto lililonse palokha ndikupeza mayankho ake ndi momwe mavutowo angathere.
female
ndikubweretsa mnyumba ya malamulo kuti boma litolemo zomwe likuona kuti ndizothandiza. Dziko la Malawi likudutsa munyengo zovuta zomwe zambiri sizikuyenda
ndikubweretsa mnyumba ya malamulo kuti boma litolemo zomwe likuona kuti ndizothandiza. Dziko la Malawi likudutsa munyengo zovuta zomwe zambiri sizikuyenda
female
Monga kukwera kwa mitengo ya katundu, kusowa kwa mafuta komanso kugwa kwa ndalama ya kwacha ndikusowa kwa ndalama za kunja zomwe kukupangitsa kuti boma ndi makampani azilephera kuitanitsa katundu kunja

koma omenyera ufulu anthu ogula katundu a John Kapito, ati izi zikuchitika chifukwa utsogoleri kumbali yotsutsa boma,
koma omenyera ufulu anthu ogula katundu a Joni Kapito, ati izi zikuchitika chifukwa utsogoleri kumbali yotsutsa boma,
female
sukuwoneka ndiye boma nalo likupanga zinthu pozindikira kuti palibe olitsutsa kapena kulidzudzula. Iwo ati mwachitsanzo, momwe njala yayambira kuvutamu
sukuwoneka ndiye boma nalo likupanga zinthu pozindikira kuti palibe olitsutsa kapena kulidzudzula. Iwo ati mwachitsanzo, momwe njala yayambira kuvutamu
female
Otsutsa amayenera kuitana boma kuti awonere limodzi zoyenera kuchita, koma mmalo mwake angotaya nthawi nkulankhula
Otsutsa amayenera kuitana boma kuti awonere limodzi zoyenera kuchita, koma mmalo mwake angotaya nthawi nkulankhula
female
kenako nkukhalanso chetee osaonetsa khumbo lenileni lofuna kuthandiza ndi vuto lomwe lilipo.
kenako nkukhalanso chetee osaonetsa khumbo lenileni lofuna kuthandiza ndi vuto lomwe lilipo.
female
Iwo ati mpata wawotsutsa wozigulitsa ngati boma lachiyembekezo ndiwomwe ukutsukulizika mkukhala chete kwawo, ndipo achenjeza kuti akapitiriza momwe akuchitira, adzavutika kuzigulitsa kwake.
Iwo ati mpata wawotsutsa wozigulitsa ngati boma lachiyembekezo ndiwomwe ukutsukulizika mkukhala chete kwawo, ndipo achenjeza kuti akapitiriza momwe akuchitira, adzavutika kuzigulitsa kwake.
female
Pa maliro a John Tembo sabata yatha, mmodzi mwa mkhala kale pa ndale, a Brown Mpinganjira, adayamikira kuti panthawi yawo ya a Tembo
Pa maliro a Joni Tembo sabata yatha, mmodzi mwa mkhala kale pa ndale, a Burawuni Mpinganjira, adayamikira kuti panthawi yawo ya a Tembo
female
mbali yotsutsa inali ya mphamvu ndipo ithandiza boma la nthawiyo la Bingu Wa Mutharika liyende bwino
mbali yotsutsa inali ya mphamvu ndipo ithandiza boma la nthawiyo la Bingu Wa Mutharika liyende bwino
female
A Mpinganjira adati chifukwa chakuchilimika kwa mbali yotsutsa nthawiyo, boma silimapanga zobwerera mmbuyo mpaka amalawi anayamikira ulamuliro wa Bingu Wa Mutharika wa term yawo yoyamba
A Mpinganjira adati chifukwa chakuchilimika kwa mbali yotsutsa nthawiyo, boma silimapanga zobwerera mmbuyo mpaka amalawi anayamikira ulamuliro wa Bingu Wa Mutharika wa teremu yawo yoyamba
female
chifukwa chamomwe otsutsa amagwirira ntchito yawo. koma mtsogoleri wa mbali yotsutsa boma a Kondwani Namkhumwa, imangosonyeza kuti akuyankhulapo mmene tilili kuyesa kuti timve maganizo awo pa zomwe akadaulowo adanena

Koma magulu osiyansiyana akhala akudzudzula mbali yotsutsa boma makamaka chipani cha Democratic Progressive chomwe nchachikulu kotsutsako kuti chikutaya nthawi ndi mikangano ya mkatikati mwa chipani
Koma magulu osiyansiyana akhala akudzudzula mbali yotsutsa boma makamaka chipani cha Dimokiratiki Purogiresivi chomwe nchachikulu kotsutsako kuti chikutaya nthawi ndi mikangano ya mkatikati mwa chipani
female
Pakati pa usiku wa lachitatu sabata yatha, ndalama ya kwaca idatsika mphamvu ndi 44 kwacha pa 100 kwacha iliyonse. Izi zachititsa kuti mitengo yakatundu ikwere zimene zikufinya amalawi.
Pakati pa usiku wa lachitatu sabata yatha, ndalama ya kwaca idatsika mphamvu ndi fote-folo kwacha pa wani handiredi kwacha iliyonse. Izi zachititsa kuti mitengo yakatundu ikwere zimene zikufinya amalawi.
female
Amalawi akhala akupereka nkhawa ndi kugwa kwa kwacha komanso ndikukwera kwa mtengo wa katundu makamaka feteleza pa nyengo ino pamene dziko likulowa nyengo ya dzinja
Amalawi akhala akupereka nkhawa ndi kugwa kwa kwacha komanso ndikukwera kwa mtengo wa katundu makamaka feteleza pa nyengo ino pamene dziko likulowa nyengo ya dzinja
female
ena mwa amalawi omwe amayankhula poyera za nkhawa zawo amadzudzula a president a Luzarus Chakewra kuti akuyendayenda kwambiri
ena mwa amalawi omwe amayankhula poyera za nkhawa zawo amadzudzula a purezidenti a Lazarasi Chakewra kuti akuyendayenda kwambiri
female
Zomwe iwo amati zikutha ndalama za kunja zomwe bwezi boma likugulira katundu yemwe amachokera kunja monga feterezayo
Zomwe iwo amati zikutha ndalama za kunja zomwe bwezi boma likugulira katundu yemwe amachokera kunja monga feterezayo
female
polankhula ku mtundu wa amalawi, atachoka kunja usiku lachitatu, a Chakwera adatambasula mfundo zotupitsira ndalama za boma
polankhula ku mtundu wa amalawi, atachoka kunja usiku lachitatu, a Chakwera adatambasula mfundo zotupitsira ndalama za boma
femalo
zomwe adalonjeza kuti zigwira ntchito yogula fetereza ndi chakudya kuti anthu asakhale ndi njala
zomwe adalonjeza kuti zigwira ntchito yogula fetereza ndi chakudya kuti anthu asakhale ndi njala
female
Ndalama zomwe tipulumutse pa ndondomekoyi yomwe takonza tiyigwiritsa ntchito pogula feteleza ndi chakudya kuti anthu paliponse mdziko muno akhale ndi chakudya chokwanira. Adatero a Chakwera.
Ndalama zomwe tipulumutse pa ndondomekoyi yomwe takonza tiyigwiritsa ntchito pogula feteleza ndi chakudya kuti anthu paliponse mdziko muno akhale ndi chakudya chokwanira. Adatero a Chakwera.
female
mwa mfundo zina zopulumutsira ndalamazo, a Chakwera ati adula maulendo awo onse kuyambira ulendo womwe analinawo kumapeto a mwezi uno wokakambirana zokhudza kusintha kwa nyengo
mwa mfundo zina zopulumutsira ndalamazo, a Chakwera ati adula maulendo awo onse kuyambira ulendo womwe analinawo kumapeto a mwezi uno wokakambirana zokhudza kusintha kwa nyengo
female
Iwo adatinso akuluakulu a boma aziyenda pogwiritsa ntchito ndalama za boma, pokhapokha iwo akawuzidwa zifukwa za ulendowo ndipo akawona kuti ndizofunika kwambiri azipereka okha chilolezo
Iwo adatinso akuluakulu a boma aziyenda pogwiritsa ntchito ndalama za boma, pokhapokha iwo akawuzidwa zifukwa za ulendowo ndipo akawona kuti ndizofunika kwambiri azipereka okha chilolezo
female
pachifukachi nduna zonse komanso akuluakulu ena aboma omwe adapita kale kunja pandalama za boma akuyenera kubwerako pompano. Adatero a Chakwera.
pachifukachi nduna zonse komanso akuluakulu ena aboma omwe adapita kale kunja pandalama za boma akuyenera kubwerako pompano. Adatero a Chakwera.
female
Iwo adalamulanso kuti nduna zonse ndi akuluakulu ena a mboma omwe amalandira mafuta a galimoto, tsopano azingodalira theka la mafuta omwe amalandira
Iwo adalamulanso kuti nduna zonse ndi akuluakulu ena a mboma omwe amalandira mafuta a galimoto, tsopano azingodalira theka la mafuta omwe amalandira
female
poyankha nkhawa yoti zinthu zakwera mwadzidzidzi anthu asadakonzekera komanso ndalama zomwe amalandira zidakali zochepa,
poyankha nkhawa yoti zinthu zakwera mwadzidzidzi anthu asadakonzekera komanso ndalama zomwe amalandira zidakali zochepa,
female
a Chakwera adati, alamula nduna yaza chuma, a Simplex Chithyola Banda kuti awunike zinthu zingapo
a Chakwera adati, alamula nduna yaza chuma, a Simpulekisi Chithyola Banda kuti awunike zinthu zingapo
female
Ndawuza nduna yaza chuma, kuti pomwe mkunika budget kuli mkati, ayikemo gawo lothandizira a business zing'onozing'ono.
Ndawuza nduna yaza chuma, kuti pomwe mkunika bajeti kuli mkati, ayikemo gawo lothandizira a bizinesi zing'onozing'ono.
female
Awunike malipiro a anthu ogwira ntchito mboma komanso misonkho yomwe anthu amapereka kuchoka ku malipiro awo. Anatero a Chakwera.
Awunike malipiro a anthu ogwira ntchito mboma komanso misonkho yomwe anthu amapereka kuchoka ku malipiro awo. Anatero a Chakwera.
female
Iwo amalankhula zonsezi patangotha ola limodzi, akuluakulu a International Monetary Fund atalengeza kuti tsopano dziko la malawi likhodza kuyambiranso kulandira thandizo lake.
Iwo amalankhula zonsezi patangotha ola limodzi, akuluakulu a Intanashono Manitare Fandi atalengeza kuti tsopano dziko la malawi likhodza kuyambiranso kulandira thandizo lake.
female
potsatira izi, a Chakwera adati, maiko ndi mabungwe osiyanasiyana omwe adasiya kuthandiza pa budget ya malawi, ayamba kulonjeza kuti ayambiranso kuthandizapo.
potsatira izi, a Chakwera adati, maiko ndi mabungwe osiyanasiyana omwe adasiya kuthandiza pa bajeti ya malawi, ayamba kulonjeza kuti ayambiranso kuthandizapo.
female
papita zaka pafupifupi 10 maikowo chisiyireni kuthandiza malawi kaamba kamomwe maboma apitawo amkayendetsera nkhani za chuma, ndipo a IMF idayitsa thandizo ku malawi mu 2020.
papita zaka pafupifupi teni maikowo chisiyireni kuthandiza malawi kaamba kamomwe maboma apitawo amkayendetsera nkhani za chuma, ndipo a aye emu efu idayitsa thandizo ku malawi mu tuwente tuwente.
female
chifukwa boma lapitalo lidapereka malipoti a bodza ku bungwelo. koma a Chakwera adati athana ndi akuluakulu onse
chifukwa boma lapitalo lidapereka malipoti a bodza ku bungwelo. koma a Chakwera adati athana ndi akuluakulu onse
female
amene adatengapo gawo lililonse kuti dziko la malawi likapezeke mmavuto aza chuma omwe adathamangitsitsa olithandiza
amene adatengapo gawo lililonse kuti dziko la malawi likapezeke mmavuto aza chuma omwe adathamangitsitsa olithandiza
female
Izi zidayankha mafunso ena omwe kadaulo paza chuma a Christopher Mbukwa adatambasulira Tamvani mmawa wa lachitatu a Chakwera akuyembekezeka kuyankhulapo madzulo ake
Izi zidayankha mafunso ena omwe kadaulo paza chuma a Khirisitofa Mbukwa adatambasulira Tamvani mmawa wa lachitatu a Chakwera akuyembekezeka kuyankhulapo madzulo ake
female
Pomwe zinthu zafika, a president akuyera kupereka chilimbikitso pankhani yokweza malipo, kuthandiza a business zing'onozing'ono kuphatikizapo alimi ang'ono ang'ono
Pomwe zinthu zafika, a purezidenti akuyera kupereka chilimbikitso pankhani yokweza malipo, kuthandiza a bizinesi zing'onozing'ono kuphatikizapo alimi ang'ono ang'ono
female
Mwachidule akuyenera kupatsa a Malawi chiyembekezo choti kugwa kwa kwacha simathero, koma kuti atero atambasule bwinobwino zomwe apange kuti zitheke. Adatero A Mbukwa.
Mwachidule akuyenera kupatsa a Malawi chiyembekezo choti kugwa kwa kwacha simathero, koma kuti atero atambasule bwinobwino zomwe apange kuti zitheke. Adatero A Mbukwa.
female
koma a Chakwera atamaliza kulankhula, a Mbukwa adauza nyuzipepala ya nation kuti a president adayankha nkhani zofunika mu uthenga wawo
koma a Chakwera atamaliza kulankhula, a Mbukwa adauza nyuzipepala ya neshoni kuti a purezidenti adayankha nkhani zofunika mu uthenga wawo
female
Mmawa wa lachitatu lomwelo, mfumu yaikulu Mwankhulukira ya ku Rumphi, inati anthu ali ndi nkhawa yaikulu makamaka pa nkhani ya feteleza.
Mmawa wa lachitatu lomwelo, mfumu yaikulu Mwankhulukira ya ku Rumphi, inati anthu ali ndi nkhawa yaikulu makamaka pa nkhani ya feteleza.
female
Yemwe tsopano adafika pa 107,000 kwacha boma litachepetsanso chiwerengero cha opindula mu AIP
Yemwe tsopano adafika pa wani handiredi andi seveni sauzandi kwacha boma litachepetsanso chiwerengero cha opindula mu eayepi
female
Apapa akonzepo chifukwa ngakhale mu AIP mavuto ayamba kale. Anthu omwe amakagula feteleza wa AIP ku Muhuju muno mu Rumphi,
Apapa akonzepo chifukwa ngakhale mu eayepi mavuto ayamba kale. Anthu omwe amakagula feteleza waeayepi ku Muhuju muno mu Rumphi,
female
abwerera akuti network pomwe ena maina sakuoneka. Adatero a Mwankhulukira. Koma apa za kufewa kwa IMF, mkulu wa bungwe la akadaulo pa zachuma,
abwerera akuti netiweki pomwe ena maina sakuoneka. Adatero a Mwankhulukira. Koma apa za kufewa kwa aye emu efu, mkulu wa bungwe la akadaulo pa zachuma,
female
La economics Association of Malawi (ECAM), a Betchani Tcheleni, adati mpofunika kusamala kwambiri kuti thandizo ngati limeneli lisathawenso.
La ikonomikisi Asosiyeshoni ofu Malawi (ikamu), a Betchani Tcheleni, adati mpofunika kusamala kwambiri kuti thandizo ngati limeneli lisathawenso.
female
Mwazina iwo adati mkofunika kutsatira ndondomeko zopulumutsira ndalama, makamaka za kunja, podula maulendo ena omwe siwofunikira kwambiri
Mwazina iwo adati mkofunika kutsatira ndondomeko zopulumutsira ndalama, makamaka za kunja, podula maulendo ena omwe siwofunikira kwambiri
female
komanso kuwonetsetsa kuti pomwe ndalama zikhodza, kupulumutsidwa mpata wotero ukugwira ntchito
komanso kuwonetsetsa kuti pomwe ndalama zikhodza, kupulumutsidwa mpata wotero ukugwira ntchito
female
Mgwirizano wa mabungwe omenyera ufulu wa anthu la Human Rights Defendants Cualission (HRDC), nalo latulutsa kalata yake yoyamikira ndondomeko zomwe a Chakwera adatambasula
Mgwirizano wa mabungwe omenyera ufulu wa anthu la Humani Rayitsi Difendantsi Kualishoni (ECHI ARA DISI), nalo latulutsa kalata yake yoyamikira ndondomeko zomwe a Chakwera adatambasula
female
Ndondomeko zimenezija nzopereka chiyembekezo kwa a Malawi, koma poti nthawi zina chimavuto nkukwaniritsa. a president akhazikitse Commission ya kalondilondo pa zomwe anena.
Ndondomeko zimenezija nzopereka chiyembekezo kwa a Malawi, koma poti nthawi zina chimavuto nkukwaniritsa. a purezidenti akhazikitse Komishoni ya kalondilondo pa zomwe anena.
female
Yatero HRDC mu kalata yake. Iyo lidachenjeza boma kwacha itangogwa mphamvu kuti likuyenera lipeze njira zoti kugwa kwa kwacha kusabweretse ululu waukulu kwa anthu.
Yatero ECHI ARA DISI mu kalata yake. Iyo lidachenjeza boma kwacha itangogwa mphamvu kuti likuyenera lipeze njira zoti kugwa kwa kwacha kusabweretse ululu waukulu kwa anthu.
female
Nduna ya zachitetezo cha m’dziko, a Ken Zikhale Ngo’oma, ati pofika mchaka cha 2025, pomwe a Malawi adzaponye vote ya adindo.
Nduna ya zachitetezo cha m’dziko, a Keni Zikhale Ngo’oma, ati pofika mchaka cha tuwente tuwente fayifi, pomwe a Malawi adzaponye voti ya adindo.
female
M’Malawi aliyese oyenera kuponya vote, adzakhala ndi chiphanso cha u mzika.
M’Malawi aliyese oyenera kuponya voti, adzakhala ndi chiphanso cha u mzika.
female
Chiphanso cha umzika ndi umbono okhawo omwe anthu m’Malawi muno akhoza kuloredwa kuponya vote, koma aphungu a m’maboma akumwera, akhala akudandawula kuti m’chigawocho, zitupa zikuvuta kutuluka.
Chiphanso cha umzika ndi umbono okhawo omwe anthu m’Malawi muno akhoza kuloredwa kuponya voti, koma aphungu a m’maboma akumwera, akhala akudandawula kuti m’chigawocho, zitupa zikuvuta kutuluka.
female
A Ng’oma ati, vuto lomwe lidalipo lakuchepa mphavu kwa makina otulutsa zitupa latha, chifukwa boma lagula makina ena amakono, komaso likukonzetsa makina ena akale omwe adawonongeka.
A Ng’oma ati, vuto lomwe lidalipo lakuchepa mphavu kwa makina otulutsa zitupa latha, chifukwa boma lagula makina ena amakono, komaso likukonzetsa makina ena akale omwe adawonongeka.
female
Imeneyo isakhale nkhawa yanu, panopa tagula makina ena owonjenzera, omwe azitulutsa zitupa 2500, patsiku.
Imeneyo isakhale nkhawa yanu, panopa tagula makina ena owonjenzera, omwe azitulutsa zitupa thu sauzandi fayifi handiredi, patsiku.
female
Ndiye osakhala ndi nkhawa, chifukwa pofika 2025, aliyese ofunika chitupa, adzakhalanacho. Atero a Ng’oma.
Ndiye osakhala ndi nkhawa, chifukwa pofika tuwente tuwente fayifi, aliyese ofunika chitupa, adzakhalanacho. Atero a Ng’oma.
female
Phungu wanyumba yamalamulo ku Thyolo South West, a Chimwemwe Chikumbu, ati mmadera ambiri kummwera, anthu akuvutika kuti apangitse kapena kubwenzeretsa zitupa zakutha.
Phungu wanyumba yamalamulo ku Thyolo Soufi Wesiti, a Chimwemwe Chikumbu, ati mmadera ambiri kummwera, anthu akuvutika kuti apangitse kapena kubwenzeretsa zitupa zakutha.
female
Tikuva kuti mzigawo zina anthu akupangitsa zitupa kapena kubwenzeretsa mosavuta, koma kwathu kuno kummwera, tikumva mavuto osiyanasiyana ena osamveka nkomwe.
Tikuva kuti mzigawo zina anthu akupangitsa zitupa kapena kubwenzeretsa mosavuta, koma kwathu kuno kummwera, tikumva mavuto osiyanasiyana ena osamveka nkomwe.
female
Nkhawa yawo, yagwirizana ndi nkhawa ya phungu wapakati m’boma la Thyolo, a Ben Phiri, omwe adati, nthambi yopereka zitupa, imayenera kukhala ndi ma Office kufupi ndi anthu.
Nkhawa yawo, yagwirizana ndi nkhawa ya phungu wapakati m’boma la Thyolo, a Beni Phiri, omwe adati, nthambi yopereka zitupa, imayenera kukhala ndi ma Ofesi kufupi ndi anthu.
female
Aphiri ati, ndondomeko yapano, anthu akuyenera kukatenga zitupa ku Office ya bwanamkubwa, ndiye potengera mtunda wokafika kumeneko, anthu ambiri amagwa ulesi.
Aphiri ati, ndondomeko yapano, anthu akuyenera kukatenga zitupa ku Ofesi ya bwanamkubwa, ndiye potengera mtunda wokafika kumeneko, anthu ambiri amagwa ulesi.
female
Bwanji osakhanzikitsa ma office kwa ma T/A, kapena mafumu akuluakulu, kuti anthu azikatengera zitupa kumeneko?
Bwanji osakhanzikitsa ma ofesi kwa ma tiye, kapena mafumu akuluakulu, kuti anthu azikatengera zitupa kumeneko?
female
Nthawi zinatu zitupa zimatuluka, koma munthu wakumudzi akaganizira mayendedwe, pamavuta. Atero a Phiri.
Nthawi zinatu zitupa zimatuluka, koma munthu wakumudzi akaganizira mayendedwe, pamavuta. Atero a Phiri.
female
A Ng’oma ati, maganizowa ndi ngoveka, koma akakambirana ku unduna, kuti awone zomwe angachite, chifukwa ndi nkhani yokhudza malamulo ndi ndondomeko za boma.
A Ng’oma ati, maganizowa ndi ngoveka, koma akakambirana ku unduna, kuti awone zomwe angachite, chifukwa ndi nkhani yokhudza malamulo ndi ndondomeko za boma.
female
Koma iwo adati, anthu omwe ali ndi zitupa zakutha, asadenkhawa, chifukwa zikuloredwa kugwira ntchito mpaka chaka cha 2026, kutanthawuza kuti akhoza kudzagwiritsa ntchito poponya vote.
Koma iwo adati, anthu omwe ali ndi zitupa zakutha, asadenkhawa, chifukwa zikuloredwa kugwira ntchito mpaka chaka cha tuwente tuwente-sikisi, kutanthawuza kuti akhoza kudzagwiritsa ntchito poponya voti.
female
Musadandawule kalikonse, palibe kusokonekera kulikonse pachisankho, woyenera kuponya vote, adzaponya amenewo ndiwo mawu anga, ndipo mukhulupirire. Atero a Ng’oma.
Musadandawule kalikonse, palibe kusokonekera kulikonse pachisankho, woyenera kuponya voti, adzaponya amenewo ndiwo mawu anga, ndipo mukhulupirire. Atero a Ng’oma.
female
Mneneri wabungwe loyendetsa chisankho la MEC a Sangwani Mwafulirwa, ati bungwero lidzapereka mpata ofanana kwa aliyese, yemwe akuyenera kudzaponya vote, osatengera boma kapena chigawo.
Mneneri wabungwe loyendetsa chisankho la MEKI a Sangwani Mwafulirwa, ati bungwero lidzapereka mpata ofanana kwa aliyese, yemwe akuyenera kudzaponya voti, osatengera boma kapena chigawo.
female
Thupi la mphangala pandale a John Tembo, lidalowa m’manda lachitatu, kumudzi kwawo kwa Kaphala, kwa T/A Kachere ku Dedza.
Thupi la mphangala pandale a Joni Tembo, lidalowa m’manda lachitatu, kumudzi kwawo kwa Kaphala, kwa tiye Kachere ku Dedza.
female
Pamwambo womwe udakusira pamodzi andale, amipingo, mafumu, ogwirantchito m’boma ndi a Malawi onse.
Pamwambo womwe udakusira pamodzi andale, amipingo, mafumu, ogwirantchito m’boma ndi a Malawi onse.
female
Maliro awo adalandira sawatcha ya a silirikali ankhondo, pamwamba pa matamando ndi litaniya za mbiriyawo, ngati munthu amene adatenga gawo lalikulu potukula ndale ndi chuma cha dziko la Malawi.
Maliro awo adalandira sawatcha ya a silirikali ankhondo, pamwamba pa matamando ndi litaniya za mbiriyawo, ngati munthu amene adatenga gawo lalikulu potukula ndale ndi chuma cha dziko la Malawi.
famale
Mwambowo udayendetsedwa ndi asirikali, ndipo adapatsa thupi la aTembo ulemu wowomba mfuti katatu, komaso lipenga la ulemu, losonyeza kuvomereza ntchito zawo m’dziko muno.
Mwambowo udayendetsedwa ndi asirikali, ndipo adapatsa thupi la aTembo ulemu wowomba mfuti katatu, komaso lipenga la ulemu, losonyeza kuvomereza ntchito zawo m’dziko muno.
female
Mbendera yaboma yomwe adakutanayo bokosi lamalemu a Tembo, idaperekedwa kwa mwana wawo, John Tembo junior, kuti ikhale chikumbutso cha malemu bambo awo.
Mbendera yaboma yomwe adakutanayo bokosi lamalemu a Tembo, idaperekedwa kwa mwana wawo, Joni Tembo juniyo, kuti ikhale chikumbutso cha malemu bambo awo.
female
Mwambo wotsiriza woperekeza aTembo unachitikira pa bwalo lamasewero la Dedza komwe mbiriyawo idatamandidwa kenako kunyamuridwa ndi asirikali ankhondo ulendo wakunyumba yawo yomaliza.
Mwambo wotsiriza woperekeza aTembo unachitikira pa bwalo lamasewero la Dedza komwe mbiriyawo idatamandidwa kenako kunyamuridwa ndi asirikali ankhondo ulendo wakunyumba yawo yomaliza.
female
Kudali misozi yosatha kuchoka kwa akubanja ndowowakonda malemu a Tembo komaso nkhope zachisoni ndizakugwa zina zosakhulupirira kuti zidalidi kumwambo wotsazikana ndi tate pa ndale.
Kudali misozi yosatha kuchoka kwa akubanja ndowowakonda malemu a Tembo komaso nkhope zachisoni ndizakugwa zina zosakhulupirira kuti zidalidi kumwambo wotsazikana ndi tate pa ndale.
female
Koma m’tsogoleri wadziko lino a Lazarous Chakwera adapepesa anamalira ndi achisoni onse, powawuza kuti iyi idali nthawi yokondwerera moyo ndi ntchito za malemu a Tembo.
Koma m’tsogoleri wadziko lino a Lazarasi Chakwera adapepesa anamalira ndi achisoni onse, powawuza kuti iyi idali nthawi yokondwerera moyo ndi ntchito za malemu a Tembo.
female
Ngakhale ili nyengo yachisoni, ndinthawiso yoti, tikumbukire zabwino zomwe adachitira dziko la Malawi mu ndale, chuma ndi chitukuko.
Ngakhale ili nyengo yachisoni, ndinthawiso yoti, tikumbukire zabwino zomwe adachitira dziko la Malawi mu ndale, chuma ndi chitukuko.
female
A Tembo adali m’modzi mwa anthu omwe dziko la Malawi silingayiwale mwa changu. Adatero a Chakwera.
A Tembo adali m’modzi mwa anthu omwe dziko la Malawi silingayiwale mwa changu. Adatero a Chakwera.
female
Iwo adapempha a Malawi kuti atengere mtima wa a Tembo wolimbikira pochita zinthu, kukonda azawo, komaso yomwe adagwira ntchito yotamandika pobweretsa umodzi m’dzikomuno.
Iwo adapempha a Malawi kuti atengere mtima wa a Tembo wolimbikira pochita zinthu, kukonda azawo, komaso yomwe adagwira ntchito yotamandika pobweretsa umodzi m’dzikomuno.
female
Pothirira ndemanga pankhaniyi pocheza ndi wayilesi ya MBC pa mwambowo, mulongo wa a Tembo yemwe adapondana naye, mayi Ivy Tembo, adati malemu a Tembo adali munthu wokonda kumanga ma ubale ndi anthu.
Pothirira ndemanga pankhaniyi pocheza ndi wayilesi ya EMUBISI pa mwambowo, mulongo wa a Tembo yemwe adapondana naye, mayi Ayive Tembo, adati malemu a Tembo adali munthu wokonda kumanga ma ubale ndi anthu.
female
Kuyambira tiri ana a John Tembo, amakonda kupanga maubale, kulikonse komwe timapita ndi malemu abambo athu omwe adali abusa, a Tembo, samachedwa kupeza azawo. Adatero mayiyo.
Kuyambira tiri ana a Joni Tembo, amakonda kupanga maubale, kulikonse komwe timapita ndi malemu abambo athu omwe adali abusa, a Tembo, samachedwa kupeza azawo. Adatero mayiyo.
female
Yemwe adali mkulu wachitetezo wa a John Tembo, a William Phakamisa, nawo adati, moyo wa a John Tembo, sudzachoka mu m’tima wawo, chifukwa adali mlerakhungwa.
Yemwe adali mkulu wachitetezo wa a Joni Tembo, a Wiliyamu Phakamisa, nawo adati, moyo wa a Joni Tembo, sudzachoka mu m’tima wawo, chifukwa adali mlerakhungwa.
female
Kupatura kutsogolera chitetezo cha a Tembo, nthawi zambiri ndimawayendetsa pa galimoto, malemu a Tembo adali ndi masomphenya akulu a dzikolino, komaso chipani cha MCP.
Kupatura kutsogolera chitetezo cha a Tembo, nthawi zambiri ndimawayendetsa pa galimoto, malemu a Tembo adali ndi masomphenya akulu a dzikolino, komaso chipani cha EMUSIPI.
female
Akhalako mndende pazifukwa zandale, komaso ndimakumbukira ine, kuti adagulitsako ina mwa minda yawo kuti athandize chipani cha MCP chitavutika nthawi imeneyo chili chotsutsa. Adatero a Phakamisa.
Akhalako mndende pazifukwa zandale, komaso ndimakumbukira ine, kuti adagulitsako ina mwa minda yawo kuti athandize chipani cha EMUSIPI chitavutika nthawi imeneyo chili chotsutsa. Adatero a Phakamisa.
female
Mlembi wa chipani cha MCP a Mkaka adakhuza a Tembo ngati m’tsuko wa upangiri wandale, pachuma, pakayendetsedwe ka dziko komaso chitukuko, kotero imfa yawo idalanda dziko la Malawi kasupe wazambiri.

Ena mwa anthu omwe adagwira ntchito ndi a Tembo monga a Nicholas Dausi, omwe ndi mneneri wa chipani cha DPP a Luise Chimango,
Ena mwa anthu omwe adagwira ntchito ndi a Tembo monga a Nikolasi Dausi, omwe ndi mneneri wa chipani cha DIPIPI a Luwisi Chimango,
female
Omwe adakhalapo speaker wa nyumba ya malamulo komaso a Brown Mpinganjira, adatamanda moyo wa a Tembo.
Omwe adakhalapo sipikala wa nyumba ya malamulo komaso a Burawuni Mpinganjira, adatamanda moyo wa a Tembo.
female
A Tembo samasankha munthu ngakhale atasiyana zipani za ndale, adali munthu wokonda anzake, adatero a Dausi.
A Tembo samasankha munthu ngakhale atasiyana zipani za ndale, adali munthu wokonda anzake, adatero a Dausi.
female
Kadawulo pa zachitetezo a Loti Dzonzi, omwe adakhalapo mkulu wa police IG m’dziko muno wawunikira kuti kubwenzeretsedwa zipata za misewu, kungakhwimitse chitetezo.
Kadawulo pa zachitetezo a Loti Dzonzi, omwe adakhalapo mkulu wa polisi ayiji m’dziko muno wawunikira kuti kubwenzeretsedwa zipata za misewu, kungakhwimitse chitetezo.
female
Izi zikudza pomwe a Malawi akudzudzula a police kuti chitetezo chatsika m’dzikomuno, potsatira ma report omwe akhala akumveka a anthu ophedwa mwa nkhanza.
Izi zikudza pomwe a Malawi akudzudzula a polisi kuti chitetezo chatsika m’dzikomuno, potsatira ma lipoti omwe akhala akumveka a anthu ophedwa mwa nkhanza.
female
Kutcholedwa kwa magalimoto, komaso umbanda wa ana a masikini. Sabata yathayi, anthu atatu odziwika, adapezeka ataphedwa nkuponyedwa mmagalimoto awo.
Kutcholedwa kwa magalimoto, komaso umbanda wa ana a masikini. Sabata yathayi, anthu atatu odziwika, adapezeka ataphedwa nkuponyedwa mmagalimoto awo.
female
Komaso ophunzira ku School ya Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources LUANaR, adaphedwa nkuponyedwa mchitsime ku Dowa.
Komaso ophunzira ku Sukulu ya Lilongwe Univesite ofu Agirikacha andi Natchuro Risosesi (LUWANA), adaphedwa nkuponyedwa mchitsime ku Dowa.
female
Povomereza nkhanizo, m’neneri wa police a Peter Kalaya, adati ziwembu zonsezo zimaoneka kuti zidali zokonzekera bwinobwino, chifukwa cholinga cha a chiwembuwo chikuwoneka kuti chidali kupha.
Povomereza nkhanizo, m’neneri wa polisi a Pita Kalaya, adati ziwembu zonsezo zimaoneka kuti zidali zokonzekera bwinobwino, chifukwa cholinga cha a chiwembuwo chikuwoneka kuti chidali kupha.
female
Tikawunika momwe ziwembu zonsezo zidakhalira, tikuona kuti achiwembuwo cholinga chawo chidali kupha, ndipo tikufufuza kuti tidziwe omwe adachita chiwembucho. Adatero a Kalaya.
Tikawunika momwe ziwembu zonsezo zidakhalira, tikuona kuti achiwembuwo cholinga chawo chidali kupha, ndipo tikufufuza kuti tidziwe omwe adachita chiwembucho. Adatero a Kalaya.
female
Koma a Dzonzi adati, kupezeka kwa zipata za police mmisewu, kumapereka mantha kwa anthu omwe akufuna kupanga chiwembu, chifukwa mpata ndi malo wopangira chiwembu amasowa.
Koma a Dzonzi adati, kupezeka kwa zipata za polisi mmisewu, kumapereka mantha kwa anthu omwe akufuna kupanga chiwembu, chifukwa mpata ndi malo wopangira chiwembu amasowa.
female
A police akuyenera kuwonjenzera kupezeka kwawo m’mizinda ndi m’misewu, zipata za police, nzofunika kwambiri.
A polisi akuyenera kuwonjenzera kupezeka kwawo m’mizinda ndi m’misewu, zipata za polisi, nzofunika kwambiri.
female
Chifukwa zimathandiza kupewa ziwembu, chifukwa anthu amawopa kuti akhoza kukumana ndi a police nthawi iliyonse. Adatero a Dzonzi.
Chifukwa zimathandiza kupewa ziwembu, chifukwa anthu amawopa kuti akhoza kukumana ndi a polisi nthawi iliyonse. Adatero a Dzonzi.
female
Mabungwe omwe si aboma, zipani zotsutsa boma komaso amalawi, akhala akupempha boma kuti likhwimitse chitetezo, malo osiyanasiyana.
Mabungwe omwe si aboma, zipani zotsutsa boma komaso amalawi, akhala akupempha boma kuti likhwimitse chitetezo, malo osiyanasiyana.
female
Izi zidayzmba pomwe anthu adayamba kugawana ma kanema a anthu othyola magalimoto, anthu ovulazidwa ndi ana amasikini, komaso za anthu omwe aphedwa posachedwapa.
Izi zidayzmba pomwe anthu adayamba kugawana ma kanema a anthu othyola magalimoto, anthu ovulazidwa ndi ana amasikini, komaso za anthu omwe aphedwa posachedwapa.
female
Koma nduna ya chitetezo cha m’dziko a Ken Zikhale Ng’oma, adati a Malawi asadenkhawa, chifukwa chitetezo chikadali bwinobwino.
Koma nduna ya chitetezo cha m’dziko a Keni Zikhale Ng’oma, adati a Malawi asadenkhawa, chifukwa chitetezo chikadali bwinobwino.
female
Iwo adati, mantha achuluka chifukwa cha nkhani zokhudza kuphedwa kwa a Allan Witika omwe ankagwira ntchito ku company ya Coca-cola.
Iwo adati, mantha achuluka chifukwa cha nkhani zokhudza kuphedwa kwa a Alani Witika omwe ankagwira ntchito ku Kampani ya Kokakola.
female
A Agness Katengeza omwe ankagwira ntchito ku Reserve Bank of Malawi, komaso bambo yemwe adapezeka ataphedwa ku area 25, ku Lilongwe.
A Aginesi Katengeza omwe ankagwira ntchito ku Rizevu Banki ofu Malawi, komaso bambo yemwe adapezeka ataphedwa ku eriya tuwente fayifi, ku Lilongwe.
female
Mphunzitsi wa chitetezo ku Mzuzu University a Aubrey Kabisala, adati kutsika kwa chitetezo, kwayenera kukhala ndi gwero lake, lomwe boma likuyenera kufufuza bwino.
Mphunzitsi wa chitetezo ku Mzuzu Univesite a Obure Kabisala, adati kutsika kwa chitetezo, kwayenera kukhala ndi gwero lake, lomwe boma likuyenera kufufuza bwino.
female
Chilipo chomwe chachititsa. sizingangobwera ayi, koma step yoyamba nkufufuza chomwe chatsitsa dzaye, kuti zinthu zifike pamenepa, kenako nkupeza njira zokonzera vutolo. Adatero a Kabisala.
Chilipo chomwe chachititsa. sizingangobwera ayi, koma sitepu yoyamba nkufufuza chomwe chatsitsa dzaye, kuti zinthu zifike pamenepa, kenako nkupeza njira zokonzera vutolo. Adatero a Kabisala.
female
Nayo committee yowowna za chitetezo,kunyumba ya malamulo, yayitanitsa nkulu wa police ndi nthambi zina zachitetezo kuti akalongosole bwino zokhudza chitetezo cha m’dziko.
Nayo komiti yowowna za chitetezo, kunyumba ya malamulo, yayitanitsa nkulu wa polisi ndi nthambi zina zachitetezo kuti akalongosole bwino zokhudza chitetezo cha m’dziko.
female