audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Apolisi ku Dowa amanga a Joseph Nyamulani a zaka 33 chifukwa chokupha mwana wazaka 6 Mphatso Zephaniah atamugunda ndi galimoto yomwe amaziphunzitsa okha
Apolisi ku Dowa amanga a Jozefe Nyamulani a zaka fetefili chifukwa chokupha mwana wazaka sikisi Mphatso Zefaniya atamugunda ndi galimoto yomwe amaziphunzitsa okha
Female
M’neneri wapolisi ku Mponela, Macpatson Msadala, wati a Nyamulani amaziphunzitsa okha galimoto ya mtundu wa Mazda Bongo Pickup yomwe nambala yake ndi DA 10825 pa bwalo la sukulu ya Chimkoka
M’neneri wapolisi ku Mponela, Makipatisoni Msadala, wati a Nyamulani amaziphunzitsa okha galimoto ya mtundu wa Mazida Bongo Pikapu yomwe nambala yake ndi Die tenieiti twentefaifi pa bwalo la sukulu ya Chimkoka
Female
koma chifukwa chothamangitsa kwambiri galimotoyo anagunda mwanayo yemwe amayenda kunja kwa bwaloli ndipo anamupweteka kwambiri m’mutu. Chifukwa chovulala kwambiri m'mutu, mwanayo, anamwalira atangofika naye kuchipatala
koma chifukwa chothamangitsa kwambiri galimotoyo anagunda mwanayo yemwe amayenda kunja kwa bwaloli ndipo anamupweteka kwambiri m’mutu. Chifukwa chovulala kwambiri m'mutu, mwanayo, anamwalira atangofika naye kuchipatala
Female
Bungwe la Mulakho wa Alhomwe lati ndilodabwa ndi mafumu ena omwe ati sakumvetsa zakusankhidwa kwa mfumu yatsopano ya Alhomwe Paramount Chief Kaduya
Bungwe la Mulakho wa Alhomwe lati ndilodabwa ndi mafumu ena omwe ati sakumvetsa zakusankhidwa kwa mfumu yatsopano ya Alomwe palamaunti tchifi Kaduya
Female
Wapampando wa bungwe la Mulakho wa Alhomwe, a Muchanakwaye Mpuluka, walankhula izi mafumu ena atatu atauza olembankhani lachisanu kuti sakugwirizana ndi momwe akuluakulu a bungweli anasankhila mfumu yatsopanoyi
Wapampando wa bungwe la Mulakho wa Alomwe, a Muchanakwaye Mpuluka, walankhula izi mafumu ena atatu atauza olembankhani lachisanu kuti sakugwirizana ndi momwe akuluakulu a bungweli anasankhila mfumu yatsopanoyi
Female
kaamba koti ati samayenela. Koma polankhula ndi MBC, wapampando wa bungwe la Mulakho wa Alhomwe a Muchanakwaye Mpuluka ati ndi odabwa kuti mafumu amene akudandaula zankhaniyi
kaamba koti ati samayenela. Koma polankhula ndi Emubisi, wapampando wa bungwe la Mulakho wa Alomwe a Muchanakwaye Mpuluka ati ndi odabwa kuti mafumu amene akudandaula zankhaniyi
Female
anali nawo pazokambirana zomwe onse anagwirizana zosankha mfumuyi kukhala pa udindowu. A Mpuluka apemphanso mamembala ake kuti apewe kumvera anthu a ndale omwe cholinga chawo ndikuwagawanitsa
anali nawo pazokambirana zomwe onse anagwirizana zosankha mfumuyi kukhala pa udindowu. A Mpuluka apemphanso mamembala ake kuti apewe kumvera anthu a ndale omwe cholinga chawo ndikuwagawanitsa
Female
Ndizodabwitsa kuti ena mwa mafumu omwe akudandaula lero, anali nawo pa tsiku lomwe aliyense anavomereza zamfumu yatsopanoyi, ndipo tikudabwa kuti iwo akudabwa lero
Ndizodabwitsa kuti ena mwa mafumu omwe akudandaula lero, anali nawo pa tsiku lomwe aliyense anavomereza zamfumu yatsopanoyi, ndipo tikudabwa kuti iwo akudabwa lero
Female
ndipotu bungwe lathu silandale, silachipembedzo koma lachikhalidwe, choncho ife sitikufuna ena kutigawanitsa, atero a Mpuluka
ndipotu bungwe lathu silandale, silachipembedzo koma lachikhalidwe, choncho ife sitikufuna ena kutigawanitsa, atero a Mpuluka
Female
Mmodzi mwa akulu akulu omwe achotsedwa mu chipani cha DPP a Ken Msonda ati chipani cha DPP chikuzipha chokha pochotsa akuluakulu ena mchipanimu
Mmodzi mwa akulu akulu omwe achotsedwa mu chipani cha Dipipi a Keni Msonda ati chipani cha Dipipi chikuzipha chokha pochotsa akuluakulu ena mchipanimu
Female
Poyankhula atangochotsedwa mchipanimu a Msonda ati sali odabwa ndi ganizo la komiti yokhazikitsa mwambo mu chipanichi
Mmodzi mwa akulu akulu omwe achotsedwa mu chipani cha DPP a Ken Msonda ati chipani cha DPP chikuzipha chokha pochotsa akuluakulu ena mchipanimu
Female
Iwo ati chipanichi chinali chitapanga kale chiganizo chochotsa anthu moti kuwaitana ku komiti yokhazikitsa mwamboyi kunali kungokwaniritsa chabe
Iwo ati chipanichi chinali chitapanga kale chiganizo chochotsa anthu moti kuwaitana ku komiti yokhazikitsa mwamboyi kunali kungokwaniritsa chabe
Female
A Msonda ati chipanichi chalakwitsa kuchotsa anthu omwe amachifunira zabwino pa mfundo zina zolakwika
A Msonda ati chipanichi chalakwitsa kuchotsa anthu omwe amachifunira zabwino pa mfundo zina zolakwika
Female
Bungwe la Malawi Gaming and Lotteries Authority ,MAGLA lachenjeza kuti lidzamanga makolo omwe amalimbikitsa ana awo kuchita juga
Bungwe la Malawi Geming’i andi Lotalezi ofolite ,MAGILA lachenjeza kuti lidzamanga makolo omwe amalimbikitsa ana awo kuchita juga
Female
Mkulu wa bungwe la MAGLA a Rachel Mijiga wati nkuphwanya malamulo kulola mwana ochepera zaka 18 kuchita nawo masewerowa
Mkulu wa bungwe la MAGILA a Recho Mijiga wati nkuphwanya malamulo kulola mwana ochepera zaka eitini kuchita nawo masewerowa
Female
A Mijiga anena izi lachisanu, pa mwambo odzala mitengo ku Lilongwe omwe inakonza ndi khonsolo ya Lilongwe
A Mijiga anena izi lachisanu, pa mwambo odzala mitengo ku Lilongwe omwe inakonza ndi khonsolo ya Lilongwe
Female
Bungwe la MAGLA ndi bungwe lomwe limaonetsetsa kuti anthu komanso makampani akutsatira malamulo a juga. Unduna owona za madzi wati mtsinje wa Naphende m'boma la Phalombe ukhoza kusefukira
Bungwe la MAGILA ndi bungwe lomwe limaonetsetsa kuti anthu komanso makampani akutsatira malamulo a juga. Unduna owona za madzi wati mtsinje wa Naphende m'boma la Phalombe ukhoza kusefukira
Female
zomwe zikupereka chiopsezo kwa anthu okhala m'madera ozungulira mtsinjewu. Izi zadza kutsatira kukwera kwa madzi mumtsinjewu omwe anawunikidwa pa mlatho wa Nankhanamba
Female zomwe zikupereka chiopsezo kwa anthu okhala m'madera ozungulira mtsinjewu.Izi zadza kutsatira kukwera kwa madzi mumtsinjewu omwe anawunikidwa pa mlatho wa Nankhanamba
Female
Mtsinjewu umadutsa m'midzi ya Likatchale, Tibu, Mwandawala, Wanye, Hammerton, Nampinga, Nandiwa komanso Phaloni
Mtsinjewu umadutsa m'midzi ya Likatchale, Tibu, Mwandawala, Wanye, Hamatoni, Nampinga, Nandiwa komanso Phaloni
Female
Mkulu woyang’anira zokhudza madzi mu undunawu, a James Chitete, wachenjeza anthu okhala madera ozungulira mtsinjewu zakusefukira kwa madzi m’maderawa
Mkulu woyang’anira zokhudza madzi mu undunawu, a Jamusi Chitete, wachenjeza anthu okhala madera ozungulira mtsinjewu zakusefukira kwa madzi m’maderawa
Female
Oyimba Nyimbo za Uzimu Evance Meleka, watulutsa nyimbo imene ikukhuza imfa ya oyimba odziwika bwino Katelele Ching'oma
Oyimba Nyimbo za Uzimu Evansi Meleka, watulutsa nyimbo imene ikukhuza imfa ya oyimba odziwika bwino Katelele Ching'oma
Female
Nyimbo-yi yomwe ikudziwika kuti "Bwanji Simunanene" Muli uthenga odandaula za kumwalira kwa oyimba ena monga Atoth Manje ndi Thomas Chibade
Nyimbo-yi yomwe ikudziwika kuti "Bwanji Simunanene" Muli uthenga odandaula za kumwalira kwa oyimba ena monga Atoti Manje ndi Thomasi Chibade
Female
Ching'oma wamwalira dzulo ku chipatala cha Kamuzu Central mu mzinda wa Lilongwe atangodwala kwa nthawi yochepa. Pangodutsa miyezi Iwiri ndi sabata ziwiri zokha pamene oyimba onsewa atsikira kuli chete
Ching'oma wamwalira dzulo ku chipatala cha Kamuzu sentilo mu mzinda wa Lilongwe atangodwala kwa nthawi yochepa. Pangodutsa miyezi Iwiri ndi sabata ziwiri zokha pamene oyimba onsewa atsikira kuli chete
Female
Apolisi m’boma la Balaka amanga anthu awiri kaamba kowaganizira kuti anapha komanso kuba m'mudzi wa Sona m'bomalo
Apolisi m’boma la Balaka amanga anthu awiri kaamba kowaganizira kuti anapha komanso kuba m'mudzi wa Sona m'bomalo
Female
Oganiziridwawa ndi a Precious Salamba a zaka 21 komanso a Enock Tonto Wonderford a zaka 20 omwe anapha a Gerald M'manjamwada ndi akazi awo a Irene Nankhanga
Oganiziridwawa ndi a Puleshasi Salamba a zaka twentewani komanso a Inoki Tonto Wandafodi a zaka twente omwe anapha a Jeladi M'manjamwada ndi akazi awo a Ayilini Nankhanga
Female
omwenso panthawiyo anawabera katundu wam'nyumba. Apolisi ndi achipatala omwe anapita kumaloku, anatsimikiza kuti anthuwo anamwalira kaamba kotaya magazi ambiri chifukwa chokhapidwa
omwenso panthawiyo anawabera katundu wam'nyumba. Apolisi ndi achipatala omwe anapita kumaloku, anatsimikiza kuti anthuwo anamwalira kaamba kotaya magazi ambiri chifukwa chokhapidwa
Female
Apolisi atapanga kafukufuku wawo, anapeza katundu yemwe anabedwayo monga, makanema awiri, ndi zinthu zina zambiri
Apolisi atapanga kafukufuku wawo, anapeza katundu yemwe anabedwayo monga, makanema awiri, ndi zinthu zina zambiri
Female
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati apitiliza kugwira ntchito za chitukuko mosayang'ana mtundu ngakhale anthu ena akhala akunamiza anthu kuti boma lake likusala anthu amtundu wa Chilhomwe
Mtsogoleri wa dziko lino Dokota Lazalasi Chakwera wati apitiliza kugwira ntchito za chitukuko mosayang'ana mtundu ngakhale anthu ena akhala akunamiza anthu kuti boma lake likusala anthu amtundu wa Chilomwe
Female
Dr Chakwera ati boma lakhazikitsa ntchito zosiyanasiyana zomwe zikupindulira aliyense kuphatikizapo anthu omwe akuyakhula izi
Dokota Chakwera ati boma lakhazikitsa ntchito zosiyanasiyana zomwe zikupindulira aliyense kuphatikizapo anthu omwe akuyakhula izi
Female
Dr Chakwera ati maiko ndi mabungwe ayambaso kuthandiza dziko lino zomwe zachititsa kuti chuma cha dziko lino chiyambenso kuyenda bwino
Dokota Chakwera ati maiko ndi mabungwe ayambaso kuthandiza dziko lino zomwe zachititsa kuti chuma cha dziko lino chiyambenso kuyenda bwino
Female
Nduna ya Zamalimidwe a Sam Kawale yapempha achinyamata ndi amayi kuti atenge mwai wa ndalama za AGCOM kuti athetse umphawi ndikuthandiza pa chitukuko cha dziko lino
Nduna ya Zamalimidwe a Samu Kawale yapempha achinyamata ndi amayi kuti atenge mwai wa ndalama za AGIKOMU kuti athetse umphawi ndikuthandiza pa chitukuko cha dziko lino
Female
Ndunayi yanena izi mmudzi mwa Manasi, Mfumu yaikulu Ngolongoliwa komwe anakayendera Mtengowamwai Producers and Marketing Cooperative
Ndunayi yanena izi mmudzi mwa Manasi, Mfumu yaikulu Ngolongoliwa komwe anakayendera Mtengowamwai Pulojusazi and Maketing’I kopeletivi
Female
Gululi linapeza ndalama pafupifupi K75 miliyoni kwacha kuchokera ku AGCOM ndipo akupanga ulimi wa tomato, komanso akwanitsa kugula galimoto
Gululi linapeza ndalama pafupifupi sevente eiti miliyoni kwacha kuchokera ku AGIKOMU ndipo akupanga ulimi wa tomato, komanso akwanitsa kugula galimoto
Female
Iwo akugwiritsa ntchito nyumba zopangiramo ulimi wa nthilira, Green Houses ndipo akupeza phindu loposa K150 miliyoni pa chaka
Iwo akugwiritsa ntchito nyumba zopangiramo ulimi wa nthilira, gilini hausezi ndipo akupeza phindu loposa wanihandede andi fifite miliyoni kwacha pa chaka
Female
Anthu odzadzidwa ndi chisoni akhamukira ku nyumba ya chisoni ya chipatala cha Kamuzu Central komwe akuchitira mwambo otenga thupi la malemu Katelele Ching'oma yemwe wamwalira usiku wathawu atadwala kwakanthawi kochepa
Anthu odzadzidwa ndi chisoni akhamukira ku nyumba ya chisoni ya chipatala cha Kamuzu sentilo komwe akuchitira mwambo otenga thupi la malemu Katelele Ching'oma yemwe wamwalira usiku wathawu atadwala kwakanthawi kochepa
Female
Ena mwa akuluakulu omwe ali nawo pamwambowu ndi mkulu wa bungwe loyang'anira oyimba m'dziko muno a Vita Chirwa, komanso akatswiri oyimba akale Billy Kaunda, Francis Molisiyo, ndi Anthony Dumba
Ena mwa akuluakulu omwe ali nawo pamwambowu ndi mkulu wa bungwe loyang'anira oyimba m'dziko muno a Vita Chirwa, komanso akatswiri oyimba akale Bile Kaunda, Fulansisi Molisiyo, ndi Anthone Dumba
Female
M'mawu ake a Chirwa ati a Katelele anali oyimba waluso kwambiri ndipo ati dziko lino liwasowa kaamba ka kuthekera kwawo kosunga chikhalidwe kudzera munyimbo zawo
M'mawu ake a Chirwa ati a Katelele anali oyimba waluso kwambiri ndipo ati dziko lino liwasowa kaamba ka kuthekera kwawo kosunga chikhalidwe kudzera munyimbo zawo
Female
Thupi la Katelele likuyembekezeka kulowa m'manda lachisanu kumudzi kwawo m'boma la Nsanje
Thupi la Katelele likuyembekezeka kulowa m'manda lachisanu kumudzi kwawo m'boma la Nsanje
Female
Katswiri pa utsogoleri ndi nkhani za ufulu, Undule Mwakasungula wati ndi okhutira ndi mmene Prezidenti Dr Lazarus Chakwera ndi boma lake akuyendetsera chuma cha dziko lino
Katswiri pa utsogoleri ndi nkhani za ufulu, Undule Mwakasungula wati ndi okhutira ndi mmene Prezidenti Dokota Lazalasi Chakwera ndi boma lake akuyendetsera chuma cha dziko lino
Female
A Mwakasangula ayankhula izi mu chikalata chomwe atulutsa Iwo ati a Malawi akuyenela kuvomeleza
A Mwakasangula ayankhula izi mu chikalata chomwe atulutsa Iwo ati a Malawi akuyenela kuvomeleza
Female
Iwo ati a Malawi akuyenela avomeleze kuti dziko lino lakhala likudutsa mu mavuto azachuma kwa zaka zapitazi
Iwo ati a Malawi akuyenela avomeleze kuti dziko lino lakhala likudutsa mu mavuto azachuma kwa zaka zapitazi
Female
ndipo ati ndizodandaulitsa kuti ena akulowetsa ndale pamavuto omwe akanatha kuchitika pa utsogoleri wina uliwonse
ndipo ati ndizodandaulitsa kuti ena akulowetsa ndale pamavuto omwe akanatha kuchitika pa utsogoleri wina uliwonse
Female
Katswiriyu wati kubweranso kwa IMF, Kuyambanso kwa thandizo ku ndondomeko yazachuma cha dziko lino, kubwera kwa thandizo kuchokera ku mabungwe ndi maiko akunja ndi nkhani yabwino yomwe ithandize kukweza chuma cha dziko lino
Katswiriyu wati kubweranso kwa ayiemuefu, Kuyambanso kwa thandizo ku ndondomeko yazachuma cha dziko lino, kubwera kwa thandizo kuchokera ku mabungwe ndi maiko akunja ndi nkhani yabwino yomwe ithandize kukweza chuma cha dziko lino
Female
Iwo ati a Malawi, akuyenela kuyamikira zomwe boma likuchita pobwezeretsa chuma mchimake, zomwe tsopano zayamba kubereka zipatso, zinthu zomwe zaka khumi zapitazi kunalibe
Iwo ati a Malawi, akuyenela kuyamikira zomwe boma likuchita pobwezeretsa chuma mchimake, zomwe tsopano zayamba kubereka zipatso, zinthu zomwe zaka khumi zapitazi kunalibe
Female
M'modzi mwa a katswiri pankhani yoswa mingoli mdziko muno Katelele Ching'oma wamwalira atadwala kwa masiku atatu
M'modzi mwa a katswiri pankhani yoswa mingoli mdziko muno Katelele Ching'oma wamwalira atadwala kwa masiku atatu
Female
Poyankhula ndi MBC m'mawa wa lero, Moses Makawa, yemwe anali mnzake waponda apa nane mpondepo wati Katelele amavutika ndi nthenda ya mmimba nthawi zambiri
Poyankhula ndi Memubisi m'mawa wa lero, Mozesi Makawa, yemwe anali mnzake waponda apa nane mpondepo wati Katelele amavutika ndi nthenda ya mmimba nthawi zambiri
Female
Amadwala inde koma masiku atatu apitawa ndi pomwe anagonekedwa pa Kamuzu Central kuchoka pachipatala cha Chinkhoma komwe anali. Lero ndi lomwe watisiya m'baleyu, watero Makawa
Amadwala inde koma masiku atatu apitawa ndi pomwe anagonekedwa pa Kamuzu sentilo kuchoka pachipatala cha Chinkhoma komwe anali. Lero ndi lomwe watisiya m'baleyu, watero Makawa
Female
Malinga ndi a Makawa, Katelele wasiya mkazi ndi ana atatu. Pakadali pano sizikudziwika komwe akayike zovutazi kaamba koti malemuyi amakhala ku Dedza koma kwawo ndi ku Nsanje
Malinga ndi a Makawa, Katelele wasiya mkazi ndi ana atatu. Pakadali pano sizikudziwika komwe akayike zovutazi kaamba koti malemuyi amakhala ku Dedza koma kwawo ndi ku Nsanje
Female
Soldier Lucius Banda yemwe ndi mlangizi wa mtsogoleri wadziko lino pankhani za luso walangiza achinyamata aluso omwe alandira ndalama (Royalties)
Soja lusiyasi Banda yemwe ndi mlangizi wa mtsogoleri wadziko lino pankhani za luso walangiza achinyamata aluso omwe alandira ndalama (Loyotezi)
Female
kuchokera ku bungwe la COSOMA agwiritse bwino ntchito ndalamazi. A Banda ayankhula izi mu mnzinda wa Lilongwe bungwe la COSOMA litapereka K500 miliyoni kwa aluso
kuchokera ku bungwe la KOSOMA agwiritse bwino ntchito ndalamazi. A Banda ayankhula izi mu mnzinda wa Lilongwe bungwe la KOSOMA litapereka Faivihandiledi miliyoni kwacha kwa aluso
Female
Ndi ochepa omwe adzathe kuimba kwa zaka 30 ngati ife ndikumapindulabe ndi luso lawo. Ife takalamba
Ndi ochepa omwe adzathe kuimba kwa zaka fete ngati ife ndikumapindulabe ndi luso lawo. Ife takalamba
Female
chomwe ndingawapemphe ndi choti agwiritse bwino ntchito ndalamazi poyamba ma bizinesi osiyanasiyana, atero a Soldier
chomwe ndingawapemphe ndi choti agwiritse bwino ntchito ndalamazi poyamba ma bizinesi osiyanasiyana, atero a Soja
Female
COSOMA yapereka ndalama zosachepera K500 miliyoni kwacha kwa oyimba, olemba mabuku, ochita zisudzo ndi ojambula makanema
KOSOMA yapereka ndalama zosachepera Faivihandiledi miliyoni kwacha kwa oyimba, olemba mabuku, ochita zisudzo ndi ojambula makanema
Female
Mkulu woona Zaumoyo m'boma la Nsanje Dr Gilbert Chapweteka walimbikitsa anthu m'bomali kuti apitilize kutsatira njira zopewera matenda a COVID-19 monga kusamba mmanja
Mkulu woona Zaumoyo m'boma la Nsanje Dokota Gilibati Chapweteka walimbikitsa anthu m'bomali kuti apitilize kutsatira njira zopewera matenda a COVIDI-Naintini monga kusamba mmanja
Female
Izi zikutsatira kupezeka kwa banja lina la anthu asanu ndi m'modzi, 6 lomwe lapezeka ndi matendawa m'bomali
Izi zikutsatira kupezeka kwa banja lina la anthu asanu ndi m'modzi, sikisi lomwe lapezeka ndi matendawa m'bomali
Female
Palibe wagonokedwa kuchipatala kaamba ka matenda-wa, anthu asachite mantha, atero Dr Chapweteka
Palibe wagonokedwa kuchipatala kaamba ka matenda-wa, anthu asachite mantha, atero Dokota Chapweteka
Female
Banki yaikulu pa dziko lonse lapansi yapereka ndalama zokwana $24O million zogwilira ntchito zothandiza kulimbana ndi kusitha kwa nyengo m'dziko muno
Banki yaikulu pa dziko lonse lapansi yapereka ndalama zokwana Thuhandiledi andi fote miliyoni Dolazi zogwilira ntchito zothandiza kulimbana ndi kusitha kwa nyengo m'dziko muno
Female
Nduna ya za chuma a Simplex Chithyola Banda, atsimikiza za nkhaniyi ndipo ati ichi ndi chitsimikizo choti maiko ndi mabungwe akukhutira ndi m'mene boma tsopano likuyendetsera chuma chake
Nduna ya za chuma a Simpulekisi Chithyola Banda, atsimikiza za nkhaniyi ndipo ati ichi ndi chitsimikizo choti maiko ndi mabungwe akukhutira ndi m'mene boma tsopano likuyendetsera chuma chake
Female
Iwo ati ndalama zochuluka zikubwera m'dziko muno zomwe zithandize kwambiri kusintha chuma komanso kutukula miyoyo ya a Malawi
Iwo ati ndalama zochuluka zikubwera m'dziko muno zomwe zithandize kwambiri kusintha chuma komanso kutukula miyoyo ya a Malawi
Female
Ndalamazi singongole.Zonsezi zikuchitika kaamba ka utsogoleri wabwino wa Dr Lazarus Chakwera, ndipo chomwe chikufunika tsopano
Ndalamazi singongole.Zonsezi zikuchitika kaamba ka utsogoleri wabwino wa Dokota Lazalasi Chakwera, ndipo chomwe chikufunika tsopano
Female
ndikuti ife amene tikuwathandiza a Chakwera komanso a Malawi tonse poyendetsa dziko lino, tigwire ntchito molimbika pokwaniritsa masomphenya amenewa, atero a Chithyola Banda
ndikuti ife amene tikuwathandiza a Chakwera komanso a Malawi tonse poyendetsa dziko lino, tigwire ntchito molimbika pokwaniritsa masomphenya amenewa, atero a Chithyola Banda
Female
Nduna yowona kuti pasakhale kusiyana pakati pa akazi ndi amuna a Jean Sendeza, apempha anthu kuti agwilire ntchito limodzi pothetsa nkhanza pakati pa okalamba m'dziko muno
Nduna yowona kuti pasakhale kusiyana pakati pa akazi ndi amuna a Jini Sendeza, apempha anthu kuti agwilire ntchito limodzi pothetsa nkhanza pakati pa okalamba m'dziko muno
Female
Polankhula pa msonkhano wa atolankhani ku Lilongwe, a Sendeza anatsindika kuti aliyense kuphatikizapo okalamba ali ndi ufulu
Polankhula pa msonkhano wa atolankhani ku Lilongwe, a Sendeza anatsindika kuti aliyense kuphatikizapo okalamba ali ndi ufulu
Female
Nkhanza zomwe zachitika posachedwapa kwa amayi achikulire m’maboma a Dowa ndi Balaka ndi zokhumudwitsa chifukwa mchitidwewu unkachitika pomwe aliyense amangoonerera ndi kujambula zithunzi
Nkhanza zomwe zachitika posachedwapa kwa amayi achikulire m’maboma a Dowa ndi Balaka ndi zokhumudwitsa chifukwa mchitidwewu unkachitika pomwe aliyense amangoonerera ndi kujambula zithunzi
Female
ndi makanema popanda opulumutsa anthuwo, anatero a Sendeza. Wothandizira mkulu wapolisi yemwenso ndi wamkulu wa apolisi am'madera, Alex Simenti, wapempha anthu m’dziko muno
ndi makanema popanda opulumutsa anthuwo, anatero a Sendeza. Wothandizira mkulu wapolisi yemwenso ndi wamkulu wa apolisi am'madera, Alekisi Simenti, wapempha anthu m’dziko muno
Female
kuti ayikirepo mtima poteteza anthu okalamba komanso kukanena ku polisi akawona khalidwe lotere. Malingana ndi undunawu
kuti ayikirepo mtima poteteza anthu okalamba komanso kukanena ku polisi akawona khalidwe lotere. Malingana ndi undunawu
Female
wati kuyambira January 2023 kufikira pano, apolisi alandira milandu 78 yochitira nkhanza okalamba pomwe ena 25 anaphedwa
wati kuyambira Januwale twente twente fili kufikira pano, apolisi alandira milandu sevente eiti yochitira nkhanza okalamba pomwe ena twentefaifi anaphedwa
Female
Akuluakulu ampingo wa CCAP Blantyre Synod alonjeza kugwira ntchito ndi boma popititsa patsogolo chitukuko cha dziko lino
Akuluakulu ampingo wa sisiepi Bulantaya sinidi alonjeza kugwira ntchito ndi boma popititsa patsogolo chitukuko cha dziko lino
Female
Mlembi wankulu wa synod-yi, M'busa Anderson Juma, wanena izi pomwe komiti yatsopano ya synod-yi, imakumana ndi mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera ku Sanjika mu mzinda wa Blantyre
Mlembi wankulu wa sinodi-yi, M'busa Andasoni Juma, wanena izi pomwe komiti yatsopano ya sinodi-yi, imakumana ndi mtsogoleri wa dziko lino Dokota Lazalasi Chakwera ku Sanjika mu mzinda wa Bulantaya
Female
Reverend Juma ati iwo atsimikizira Prezidenti Chakwera kuti athandiza boma pomwe likuyesetsa kuthana ndi mavuto azachuma. Iwo ati ndiokhutira ndi zomwe boma lkuchita pothana ndi mavutowa
Reverendi Juma ati iwo atsimikizira Prezidenti Chakwera kuti athandiza boma pomwe likuyesetsa kuthana ndi mavuto azachuma. Iwo ati ndiokhutira ndi zomwe boma lkuchita pothana ndi mavutowa
Female
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera mawa akuyembekezeka kuyendera ntchito zina za chitukuko zomwe boma likugwira
Mtsogoleri wa dziko lino Dokota Lazalasi Chakwera mawa akuyembekezeka kuyendera ntchito zina za chitukuko zomwe boma likugwira
Female
m'boma la Blantyre komanso Chikwawa. Malinga ndi chikalata chofotokoza zaulendowu chomwe chasainidwa ndi mlembi mu ofesi ya Prezidenti ndi nduna, Colleen Zamba, ulendo woyendera zitukukukozi udzayamba 8 koloko m'mawa
m'boma la Bulantaya komanso Chikwawa. Malinga ndi chikalata chofotokoza zaulendowu chomwe chasainidwa ndi mlembi mu ofesi ya Prezidenti ndi nduna, Colini Zamba, ulendo woyendera zitukukukozi udzayamba eiti koloko m'mawa
Female
Tsizinamtole wina wa wazaka 27 Geoffrey Matewere wamwalira atagwidwa ndi nyetsi yamagetsi ku Monkey Bay
Tsizinamtole wina wa wazaka twente seveni Jofule Matewere wamwalira atagwidwa ndi nyetsi yamagetsi ku Monkibe
Female
M'neneri wapolisi ku Monkey Bay, Alice Sichali, watsimikiza za nkhaniyi, ponena kuti Matewere wamwalira
M'neneri wapolisi ku Monkibe, Alisi Sichali, watsimikiza za nkhaniyi, ponena kuti Matewere wamwalira
Female
pa 15 January chaka chomwe chino pamene amagwiragwira nthambo za magetsi ku parishi ya Nankhwali kwa mfumu yaikulu Nankumba
pa fifitini Januwale chaka chomwe chino pamene amagwiragwira nthambo za magetsi ku parishi ya Nankhwali kwa mfumu yaikulu Nankumba
Female
Malemuwa anali kabwerebwere pa nkhani yokuba. Mwatsoka patsikuli, anagwidwa ndi nyetsi yamagetsi pamene amafuna kuba zipangizo za magetsi za ESCOM
Malemuwa anali kabwerebwere pa nkhani yokuba. Mwatsoka patsikuli, anagwidwa ndi nyetsi yamagetsi pamene amafuna kuba zipangizo za magetsi za ESIKOMU
Female
kunja kwa parishi ya Nankhwali ndipo anapezeka atamwalira panja pa chipinda cha wansembe wina," anatero a Sichali Apolisi apempha anthu m'bomali kuti asiye kugwiragwira nthambo za ESCOM kuti apewe ngozi zoterezi
kunja kwa parishi ya Nankhwali ndipo anapezeka atamwalira panja pa chipinda cha wansembe wina," anatero a Sichali Apolisi apempha anthu m'bomali kuti asiye kugwiragwira nthambo za ESIKOMU kuti apewe ngozi zoterezi
Female
Matewere amachokera m'mudzi mwa Mwenda, mfumu yaikulu Nankumba, m'boma la Mangochi. Nduna ya Zaulimi a Sam Kawale
Matewere amachokera m'mudzi mwa Mwenda, mfumu yaikulu Nankumba, m'boma la Mangochi. Nduna ya Zaulimi a Samu Kawale
Female
apereka zipangizo za ulimi kwa magulu atatu aulimi kwa mfumu yaikulu Kuntaja m'boma la Blantyre. Maguluwa omwe mayina awo ndi Kuwala, Tafika komanso Umodzi
apereka zipangizo za ulimi kwa magulu atatu aulimi kwa mfumu yaikulu Kuntaja m'boma la Bulantaya. Maguluwa omwe mayina awo ndi Kuwala, Tafika komanso Umodzi
Female
analandira chithandizo cha ndalama kuchokera ku bungwe la Agriculture Commercialization Project ,AGCOM. Gulu la Kuwala linalandira ndalama zokwana K148 million, pomwe Tafika linalandira K46 million
analandira chithandizo cha ndalama kuchokera ku bungwe la Agilikacha komeshalayizeshoni pulojekiti, AGIKOMU. Gulu la Kuwala linalandira ndalama zokwana wanihandedi andi fote eiti miliyoni kwacha, pomwe Tafika linalandira fote sikisi miliyoni kwacha
Female
ndipo Umodzi lomwe ndi gulu la achinyamata, linalandira K32 million. Magulu onse atatu, akupanga ulimi wa soya, nyemba komanso kuweta nkhuku
ndipo Umodzi lomwe ndi gulu la achinyamata, linalandira fete thu miliyoni kwacha. Magulu onse atatu, akupanga ulimi wa soya, nyemba komanso kuweta nkhuku
Female
Zipangizo za ulimi zomwe agula ndi ndalama yomwe analandira ndi; mathirakitala, mapulawo, mafiriji komanso zipangizo zofungatira mazira, Incibators Magulu onse atatu ali ndi misika yokhazikika kale
Zipangizo za ulimi zomwe agula ndi ndalama yomwe analandira ndi; mathirakitala, mapulawo, mafiriji komanso zipangizo zofungatira mazira, Inkyubetazi Magulu onse atatu ali ndi misika yokhazikika kale
Female
Apolisi Ku Mulanje amanga a Square Valamanja mphunzitsi wa sukulu ya pulayimale yemwe akuganiziridwa kuti anathyola ndi kuba m'nyumba ya a Frank Deshani
Apolisi Ku Mulanje amanga a Sikweya Valamanja mphunzitsi wa sukulu ya pulayimale yemwe akuganiziridwa kuti anathyola ndi kuba m'nyumba ya a Fulanki Deshani
Female
M'neneri wa polisi ya Mulanje, a Innocent Moses, ati apolisi atapanga kafuku-fuku, ati anawapeza a Valamanja ndi katundu wandalama zokwana K2.8 million
M'neneri wa polisi ya Mulanje, a Inosenti Mozesi, ati apolisi atapanga kafuku-fuku, ati anawapeza a Valamanja ndi katundu wandalama zokwana thu pointi eiti miliyoni kwacha
Female
yemwe akuwaganizira kuti anaba kwa a Deshani. A Moses ati amene akuwaganizirawa sikoyamba kupalamula mlandu omwewu
yemwe akuwaganizira kuti anaba kwa a Deshani. A Mozesi ati amene akuwaganizirawa sikoyamba kupalamula mlandu omwewu
Female
ndipo ali ndi zaka 41 zakubadwa komanso amachokera m'mudzi mwa Takhiwa, mfumu yayikulu Njema, m'boma la Mulanje
ndipo ali ndi zaka fotewani zakubadwa komanso amachokera m'mudzi mwa Takhiwa, mfumu yayikulu Njema, m'boma la Mulanje
Female
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera, wasintha dzina la chipatala chachikulu cha m’boma la Phalombe ndipo chizidziwika kuti Chilembwe
Mtsogoleri wa dziko lino Dokota Lazalasi Chakwera, wasintha dzina la chipatala chachikulu cha m’boma la Phalombe ndipo chizidziwika kuti Chilembwe
Female
Dr Chakwera ati izi zili chomwechi pofuna kulemekeza m’busa John Chilembwe amene anadzipereka pofuna kukuza ntchito za chitukuko monga maphunziro ndi za umoyo
Dokota Chakwera ati izi zili chomwechi pofuna kulemekeza m’busa John Chilembwe amene anadzipereka pofuna kukuza ntchito za chitukuko monga maphunziro ndi za umoyo
Female
Mtsogoleriyu, walimbikitsanso makolo kuti azilimbikitsa ana awo kuti azilimbikira maphunziro. Dr Chakwera amayankhula pa mwambo wokumbukira m’busa John Chilembwe
Mtsogoleriyu, walimbikitsanso makolo kuti azilimbikitsa ana awo kuti azilimbikira maphunziro. Dokota Chakwera amayankhula pa mwambo wokumbukira m’busa Joni Chilembwe
Female
pa Providence Industrial Mission, PIM m'boma la Chiradzulu. nduna yamaboma ang'ono umodzi komanso chikhalidwe a Richard Chimwendo Banda apempha anthu mdziko muno
pa Pulovinsi indasitiliyo mishoni, Piayiemu m'boma la Chiradzulu. nduna yamaboma ang'ono umodzi komanso chikhalidwe a Richard Chimwendo Banda apempha anthu mdziko muno
Female
kuti asaike ndale patsogolo koma m'malo mwake agwire ntchito zotukula dziko lino mogwirizana ndi masomphenya a boma. Iwo ati boma likugwira ntchito zochuluka zachitukuko
kuti asaike ndale patsogolo koma m'malo mwake agwire ntchito zotukula dziko lino mogwirizana ndi masomphenya a boma. Iwo ati boma likugwira ntchito zochuluka zachitukuko
Female
kuphatikizapo kumanga misewu, njanji ku Nsanje, nyumba za achitetezo, milatho, zipatala poonjezera kupereka chimanga komanso ndalama za Mtukula Pakhomo kwa anthu ovutika
kuphatikizapo kumanga misewu, njanji ku Nsanje, nyumba za achitetezo, milatho, zipatala poonjezera kupereka chimanga komanso ndalama za Mtukula Pakhomo kwa anthu ovutika
Female
A Chimwendo Banda ati mwa chitsanzo, boma latsegulanso bungwe la ADMARC lomwe layamba tsopano kugulitsa chimanga kwa anthu m'dziko muno, koma anati ndi odandaula kuti mavenda akusokoneza ntchitoyi.
A Chimwendo Banda ati mwa chitsanzo, boma latsegulanso bungwe la ADIMAKI lomwe layamba tsopano kugulitsa chimanga kwa anthu m'dziko muno, koma anati ndi odandaula kuti mavenda akusokoneza ntchitoyi.
Female
Iwo apempha mafumu kuti athandize polimbana ndi mchitidwewu kuti anthu osauka apindule. Iwo anena izo pamwambo okumbukira m'busa John Chilembwe, ku PIM m'boma la Chiradzulu
Iwo apempha mafumu kuti athandize polimbana ndi mchitidwewu kuti anthu osauka apindule. Iwo anena izo pamwambo okumbukira m'busa John Chilembwe, ku Piayiemu m'boma la Chiradzulu
Female
Kampani yopanga Magetsi mdziko muno ya Electricity Generation Company EGENCO yati tsopano yamaliza ntchito yokonza makina ake a Nkula A ndi B
Kampani yopanga Magetsi mdziko muno ya Elekithilisite jeneleshoni kampane IJENKO yati tsopano yamaliza ntchito yokonza makina ake a Nkula E ndi Bi
Female
Malingana ndi chikalata chomwe atulutsa, makina onse tsopano akugwira ntchito moyenera. Kampaniyi inalengeza zoti Magetsi adzithimathima
Malingana ndi chikalata chomwe atulutsa, makina onse tsopano akugwira ntchito moyenera. Kampaniyi inalengeza zoti Magetsi adzithimathima
Female
mmadera ena kuyambira loweluka pa 13 January 2024 mpaka Lolemba 15 January 2024 pamene kampaniyi imakonza makina ake
mmadera ena kuyambira loweluka pa fetini Januwale twente twente folo mpaka Lolemba fifitini Januwale twentetwente folo pamene kampaniyi imakonza makina ake
Female
Zateremu ndiye kuti magetsi sathimathimanso monga mmene zinaliri masiku apitawa. Zithunzi zili mmusizi zikuonetsa malo omwe panali nyumba ya mayi ali pachinthunzipa yemwe nyumba yake yakokoloka
Zateremu ndiye kuti magetsi sathimathimanso monga mmene zinaliri masiku apitawa. Zithunzi zili mmusizi zikuonetsa malo omwe panali nyumba ya mayi ali pachinthunzipa yemwe nyumba yake yakokoloka
Female
kutsatira kusefukira kwa mtsinje wa Kasangadzi ku Dowa pa 13 January 2024. Tsiku linayamba bwino kwa Violet Banaba wazaka 38, ochokera mmudzi mwa Kasangadzi 2
kutsatira kusefukira kwa mtsinje wa Kasangadzi ku Dowa pa fetini Januwale twente twente folo. Tsiku linayamba bwino kwa Vayoleti Banaba wazaka fete eiti, ochokera mmudzi mwa Kasangadzi thu
Female
m'dera la mfumu yayikulu Dzoole ku Dowa koma tsikuli silinathe bwino nyengo itatembenuka ndipo mvula yamphamvu yomwe inagwa mderali inapangitsa mtsinje wa Kasangadzi kusefukira ndi kukokolora nyumba za anthu ena mderali
m'dera la mfumu yayikulu Dzoole ku Dowa koma tsikuli silinathe bwino nyengo itatembenuka ndipo mvula yamphamvu yomwe inagwa mderali inapangitsa mtsinje wa Kasangadzi kusefukira ndi kukokolora nyumba za anthu ena mderali
Female