audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Gogo Timbiri nawo ayamikira zintchito za a Ndhlozi ponena kuti masomphenya abwino omwe ali nawowa apitilize, ndipo iwo alangiza onse akufuna kuzapikisana nawo pa zisankho za 2025
Gogo Timbiri nawo ayamikira zintchito za a Zyozi ponena kuti masomphenya abwino omwe ali nawowa apitilize, ndipo iwo alangiza onse akufuna kuzapikisana nawo pa zisankho za twente twente faifi
Female
pa ma undindo wosiyana siyana kuti akonzekere kukhazikitsa fundo za chitukuko zomwe atha kuzakwanitsa
pa ma undindo wosiyana siyana kuti akonzekere kukhazikitsa fundo za chitukuko zomwe atha kuzakwanitsa
Female
Bambo Lloyd Ndhlozi ndi Mlembi wa mkulu wa Chipani cha Freedom ku chigawo cha kumpoto, chipani chomwe chikutsogozedwa ndi wachiwiri wa mtsogoleri wakale wadziko lino a Khumbo KachalI
Bambo Loyidi Zyozi ndi Mlembi wa mkulu wa Chipani cha Fulidomu ku chigawo cha kumpoto, chipani chomwe chikutsogozedwa ndi wachiwiri wa mtsogoleri wakale wadziko lino a Khumbo Kachali
Female
Iwo anatengelaponso mwayi kunena kuti chipanichi chachilimika kuti anthu ake azawatumikire mtundu wa Malawi
Iwo anatengelaponso mwayi kunena kuti chipanichi chachilimika kuti anthu ake azawatumikire mtundu wa Malawi
Female
Patangodutsa maola ochepa woyimba wamkazi Tuno atadandaula za kusakondedwa, naye Temwa Gondwe wadandaula zomwezo ndipo akudzifusa kuti Ndili kuti
Patangodutsa maola ochepa woyimba wamkazi Tuno atadandaula za kusakondedwa, naye Temwa Gondwe wadandaula zomwezo ndipo akudzifusa kuti Ndili kuti
Female
pomwe anthu ena awugogodi ayamba kumutoza. Chatsitsa dzaye kuti njovu ithyoke nyanga nchakuti, mkati mwasabatayi, Temwah yemwe ndimwini wake wa nyimbo ya Mvetsera
pomwe anthu ena awugogodi ayamba kumutoza. Chatsitsa dzaye kuti njovu ithyoke nyanga nchakuti, mkati mwasabatayi, Temwah yemwe ndimwini wake wa nyimbo ya Mvetsera
Female
yomwe anaimba limodzi ndi Zeze ndipo chaka chatha yawonongetsa anthu ndalama, anayika pa tsamba lake la fesibuku chithuzi cha mwana wake wa miyezi isanu ndi umodzi
yomwe anaimba limodzi ndi Zeze ndipo chaka chatha yawonongetsa anthu ndalama, anayika pa tsamba lake la fesibuku chithuzi cha mwana wake wa miyezi isanu ndi umodzi
Female
Apa Temwa yemwe chaka chatha wakokolora mphoto za mnanu kamba ka mayimbidwe ake apamwamba, sanadziwe kuti wadzikodolera anthu onunkha nkamwa
Apa Temwa yemwe chaka chatha wakokolora mphoto za mnanu kamba ka mayimbidwe ake apamwamba, sanadziwe kuti wadzikodolera anthu onunkha nkamwa
Female
omwe monga zimachitira ntchentche zikaona chimbudzi, anakhamukira pa tsambali ndikuyamba kulavula zakukhosi, zomunyoza woyimbayu pamodzi ndi khanda lake losalakwalo
omwe monga zimachitira ntchentche zikaona chimbudzi, anakhamukira pa tsambali ndikuyamba kulavula zakukhosi, zomunyoza woyimbayu pamodzi ndi khanda lake losalakwalo
Female
Ndemanga zina zomwe tsamba lino lawona, anthu ena anayamba kufanizira mwana wa Temwa ndi katswiri oyimba chamba cha amapiano, Zeze Kingston
Ndemanga zina zomwe tsamba lino lawona, anthu ena anayamba kufanizira mwana wa Temwa ndi katswiri oyimba chamba cha amapiano, Zeze King’isitoni
Female
ngakhale kuti awiriwa pano samamwelana madzi pazifukwa zodziwa okha. Mnyozo ngati uwu komaso zina, ndi zomwe zatutumutsa Temwa
ngakhale kuti awiriwa pano samamwelana madzi pazifukwa zodziwa okha. Mnyozo ngati uwu komaso zina, ndi zomwe zatutumutsa Temwa
Female
yemwe Lachinayi analemba pa tsamba lake la fesibuku kudandaula za kusakondedwa kwake ndi anthu ochuluka mdziko muno ndipo wafika pofusa kuti kapena zoyimbazi ayambe watenga kaye tchuthi
yemwe Lachinayi analemba pa tsamba lake la fesibuku kudandaula za kusakondedwa kwake ndi anthu ochuluka mdziko muno ndipo wafika pofusa kuti kapena zoyimbazi ayambe watenga kaye tchuthi
Female
Koma mukuti ndinalakwa chani kweni kweni , Mwina lelo mundiuze ndinvesese, Sindilimbana ndi munthu ndikabwela pa Facebook pano ndimapanga za nyimbo zanga
Koma mukuti ndinalakwa chani kweni kweni , Mwina lelo mundiuze ndinvesese, Sindilimbana ndi munthu ndikabwela pa Fesibuku pano ndimapanga za nyimbo zanga
Female
kuti mpaka mu muike mwana wanga zosamukhudza mwana achepelenji, so innocent as her mother ndapanga post just to appreciate my daughter Koma ayi ndithu ena akuipidwa nazo zimenezizi
kuti mpaka mu muike mwana wanga zosamukhudza mwana achepelenji, so inosenti azi ha mava ndapanga positi jasiti tu apulisiyeti mayi dota Koma ayi ndithu ena akuipidwa nazo zimenezizi
Female
Woyimbayu wati akudziwa kuti anthu ambiri akumupangira kaduka chifukwa choti zinthu zikumuyendera ndipo wati akudziwaso kuti anthu ambiri akupanga izi
Woyimbayu wati akudziwa kuti anthu ambiri akumupangira kaduka chifukwa choti zinthu zikumuyendera ndipo wati akudziwaso kuti anthu ambiri akupanga izi
Female
kamba koti akufunitsitsa banja lake lithe, zomwe wati sizinthu zabwino. Bwanji mumakwiya anzanu zikamawayendela ndi ufiti umenewo
kamba koti akufunitsitsa banja lake lithe, zomwe wati sizinthu zabwino. Bwanji mumakwiya anzanu zikamawayendela ndi ufiti umenewo
Female
Basi kukhosi mbeee Temwa asowe mtendele Temwa banja lake lithe Temwa ndi hule temwa this temwa that eh nakulakwilani chani, Anateloso Temwa popitilira ndi uthenga wake pa fesibuku
Basi kukhosi mbeee Temwa asowe mtendele Temwa banja lake lithe Temwa ndi hule temwa visi temwa vati eh nakulakwilani chani, Anateloso Temwa popitilira ndi uthenga wake pa fesibuku
Female
Pakadali pano masamba ambiri pa fesibuku akudzudzula chipongwe chomwe anthu akupangira oyimbayu ponena kuti izi zithakuwononga luso lomwe Temwa ali nalo
Pakadali pano masamba ambiri pa fesibuku akudzudzula chipongwe chomwe anthu akupangira oyimbayu ponena kuti izi zithakuwononga luso lomwe Temwa ali nalo
Female
kamba koti zili ndikuthekera koti atha kuyimba kudziyang’anira pansi komaso kubwelera mbuyomu pa mayimbidwe
kamba koti zili ndikuthekera koti atha kuyimba kudziyang’anira pansi komaso kubwelera mbuyomu pa mayimbidwe
Female
Chaka chatha, mtsutso unabuka pa masamba a nchezo pa nkhani yoti pakati pa Temwa ndi Zeze amene anatchukitsa mzake ndindani
Chaka chatha, mtsutso unabuka pa masamba a nchezo pa nkhani yoti pakati pa Temwa ndi Zeze amene anatchukitsa mzake ndindani
Female
zomwe zinapangitsa oyimba awiri wa kusiya kuyimbira limodzi ndipo kenaka chidani cha khoswe ndi mphaka chidayambika komaso anthu ankatsutsana kuti kodi awiriwa chinali chibwezi kapena ankangoyimbira limodzi chabe

Watiyankhulira bwino, A Malawi lekani kuika oyimba pa mpikisano, Lucius Banda watayira ka mtengo Namadingo
Watiyankhulira bwino, A Malawi lekani kuika oyimba pa mpikisano, Lusiyasi Banda watayira ka mtengo Namadingo
Female
Chiyamba kale pa maimbidwe Lucius Banda watayira ka mtengo oyimba wamakono, Patience Namadingo, poyankhula zakupsa posachedwapa koma wadzudzula anthu mdziko muno
Chiyamba kale pa maimbidwe Lusiyasi Banda watayira ka mtengo oyimba wamakono, Peshesi Namadingo, poyankhula zakupsa posachedwapa koma wadzudzula anthu mdziko muno
Female
kuti asiye mchitidwe oyika oyimba pa mpikisano. Izi zili mu uthenga omwe Banda wayika pa tsamba lake la fesibuku Lachitatu pa 31 January, 2024 momwe amayamikira mfundo zokhwima
kuti asiye mchitidwe oyika oyimba pa mpikisano. Izi zili mu uthenga omwe Banda wayika pa tsamba lake la fesibuku Lachitatu pa fetewani januwale twente twente folo momwe amayamikira mfundo zokhwima
Female
komaso zogwira ntima zomwe Namadingo anayankhula mu pologalamu ya padera pa wayilesi ya Times. Usiku wa Loweluka, pa 27 January, 2024
komaso zogwira ntima zomwe Namadingo anayankhula mu pologalamu ya padera pa wayilesi ya Taimusi. Usiku wa Loweluka, pa twente seveni Januwale Twente twente folo
Female
oyimba Namadingo amacheza ndi Brian Banda pa wayilesi ya Times ndipo mwa zina iye anafotokoza kuti kuchita bwino kwa oyimba anzake omwe atekeseka pa Malawi pakadali pano
oyimba Namadingo amacheza ndi Bulayani Banda pa wayilesi ya Taimusi ndipo mwa zina iye anafotokoza kuti kuchita bwino kwa oyimba anzake omwe atekeseka pa Malawi pakadali pano
Female
sikukuyenera kukhale chiopsezo koma chilimbikitso pa oyimba wina aliyese mdziko muno. Poyankhula za nkhaniyi, Banda yemwe ndi wa mvula za kale pa nkhani ya maimbidwe mdziko muno
sikukuyenera kukhale chiopsezo koma chilimbikitso pa oyimba wina aliyese mdziko muno. Poyankhula za nkhaniyi, Banda yemwe ndi wa mvula za kale pa nkhani ya maimbidwe mdziko muno
Female
wati mfundo zochuluka zomwe Namadingo anayankhula mu pologalamu yapaderayi, zamugwira mtima kwabasi. Nzira zembe pamayimbidweyu yemweso amadziwika ndi dzina loti Soldier
wati mfundo zochuluka zomwe Namadingo anayankhula mu pologalamu yapaderayi, zamugwira mtima kwabasi. Nzira zembe pamayimbidweyu yemweso amadziwika ndi dzina loti Soja
Female
wati yankho lomwe Namadingo anapeleka pa fuso loti kodi amaopsedwa ndi oyimba anzake omwe akuchita bwino pakadali pano omwe ndikuphatikizapo Driemo, wayankhira oyimba ochuluka
wati yankho lomwe Namadingo anapeleka pa fuso loti kodi amaopsedwa ndi oyimba anzake omwe akuchita bwino pakadali pano omwe ndikuphatikizapo Diliyemo, wayankhira oyimba ochuluka
Female
Ndakhala ndikusilira kaganizidwe ka mnyamatayu komaso kuthekera kwa kufotokoza mwaveveve pa zinthu zokhudzana ndi luso lathu la maimbidwe
Ndakhala ndikusilira kaganizidwe ka mnyamatayu komaso kuthekera kwa kufotokoza mwaveveve pa zinthu zokhudzana ndi luso lathu la maimbidwe
Female
Pakuyankhulana kwake ndi Brian Banda posachedwapa, ndiunikira funso limodzi lomwe adayankha lomwe ndikuganiza kuti adayankha kwa oyimba tonse
Pakuyankhulana kwake ndi Brulayani Banda posachedwapa, ndiunikira funso limodzi lomwe adayankha lomwe ndikuganiza kuti adayankha kwa oyimba tonse
Female
Atafunsidwa za kuchita bwino kwa Driemo kuposa kwake, iye anati kupambana kwa woimba m’modzi ndi chipambano cha oyimba onse,” haaa! Mwana iwe watiyankhila bwino zedi
Atafunsidwa za kuchita bwino Kwa Diliyemo kuposa kwake, iye anati kupambana kwa woimba m’modzi ndi chipambano cha oyimba onse,” haaa! Mwana iwe watiyankhila bwino zedi
Female
watelo Banda mu uthenga omwe anaulemba mchingerezi. Mkuluyu yemwe pano watekesa pa Malawi ndi nyimbo ya chikondi ya Umunyengerere, sanalekere pomwepa
watelo Banda mu uthenga omwe anaulemba mchingerezi. Mkuluyu yemwe pano watekesa pa Malawi ndi nyimbo ya chikondi ya Umunyengerere, sanalekere pomwepa
Female
koma kudzudzula a Malawi kuti asiye khalidwe lomawayika oyimba mdziko muno pa mpikisano zomwe wati ndizolakwoka kwambiri. A Malawi lekani kuwayika oyimba anu pa mpikisanu
koma kudzudzula a Malawi kuti asiye khalidwe lomawayika oyimba mdziko muno pa mpikisano zomwe wati ndizolakwoka kwambiri. A Malawi lekani kuwayika oyimba anu pa mpikisanu
Female
aliyense ndiwosiyana ndi nzake muzichitochito. Muwathandize ngati gulu la nkhondo kuti akwanitse kugonjetsa dziko la pansi. Zikomo Dr Namadingo
aliyense ndiwosiyana ndi nzake muzichitochito. Muwathandize ngati gulu la nkhondo kuti akwanitse kugonjetsa dziko la pansi. Zikomo Dokota Namadingo
Female
Ndikupitiliza kukudalitsa kuti upite ku malo osiyanasiyana kukagulitsa mbendera ya dziko la Malawi pa nkhani ya mayimbidwe, wateloso Banda
Ndikupitiliza kukudalitsa kuti upite ku malo osiyanasiyana kukagulitsa mbendera ya dziko la Malawi pa nkhani ya mayimbidwe, wateloso Banda
Female
Namadingo wayankhula zokhudza mayimbidwe kwa nthawi yoyamba patadutsa dzaka zisanu, ndipo pakadali pano waneneratu
Namadingo wayankhula zokhudza mayimbidwe kwa nthawi yoyamba patadutsa dzaka zisanu, ndipo pakadali pano waneneratu
Female
kuti anthu asayembekezeso kuti posachedwapa amuwonaso akuyankhula pa wayilesi pa nkhani za mayimbidwe
kuti anthu asayembekezeso kuti posachedwapa amuwonaso akuyankhula pa wayilesi pa nkhani za mayimbidwe
Female
Tsopano mayendedwe akhala wovutirapo pa msewu wa M5 pamene madzi ochuluka adula msewuwu, omwe umatchedwanso kuti Lakeshore, kamba ka mvula yamphamvu yomwe yakhala ikugwa
Tsopano mayendedwe akhala wovutirapo pa msewu wa emu faifi pamene madzi ochuluka adula msewuwu, omwe umatchedwanso kuti Lekisho, kamba ka mvula yamphamvu yomwe yakhala ikugwa
Female
Msewu umenewu waduka pa malo otchedwa Mwalawoyera kuchokera pa Salima Turn Off kupita ku Salima. Malingana ndi a Portia Kajanga omwe ndi ofalitsa nkhani za bungwe la Roads Authority
Msewu umenewu waduka pa malo otchedwa Mwalawoyera kuchokera pa Salima Thenofu kupita ku Salima. Malingana ndi a Potiya Kajanga omwe ndi ofalitsa nkhani za bungwe la Rodzi ofolite
Female
izi zili chomwechi kamba kakuti anthu ena akhala akuba zitsulo zapa mlathowo. Iwo atsimikiza kuti pakadali pano
izi zili chomwechi kamba kakuti anthu ena akhala akuba zitsulo zapa mlathowo. Iwo atsimikiza kuti pakadali pano
Female
palibe galimoto yomwe ingadutse pamalopo kamba kakuti mlathowo waonongekeratu
palibe galimoto yomwe ingadutse pamalopo kamba kakuti mlathowo waonongekeratu
Female
A Kajanga apempha anthu kuti ngati akufuna kuti agwiritse ntchito msewu umenewu akuyenera kudzera msewu wa Khwekhwelele, Golomoti ngati akufuna kupita ku Salima pamene
A Kajanga apempha anthu kuti ngati akufuna kuti agwiritse ntchito msewu umenewu akuyenera kudzera msewu wa Khwekhwelele, Golomoti ngati akufuna kupita ku Salima pamene
Female
akuchokera ku Ntcheu kapena ku Balaka. Iwo afotokozanso kuti akatswiri owona za msewu afika kale pamalopo kukonza mlathowu pofuna kuti ntchito zamayendedwezi zibwelele m’chimake
akuchokera ku Ntcheu kapena ku Balaka. Iwo afotokozanso kuti akatswiri owona za msewu afika kale pamalopo kukonza mlathowu pofuna kuti ntchito zamayendedwezi zibwelele m’chimake
Female
Awunikirenso ngati ofesi ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino ndiyofunika, watero Namiwa Malingana mkuona kwa a Sylvester Namiwa
Awunikirenso ngati ofesi ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino ndiyofunika, watero Namiwa Malingana mkuona kwa a Silivesita Namiwa
Female
yemwe ndi mkulu wa bungwe la CDEDI, ati ofesiyi ya mtsogoleri wachiwiri mdziko muno siikuwoneka ntchito yeni yeni yomwe ikugwira
yemwe ndi mkulu wa bungwe la sidi idiayi, ati ofesiyi ya mtsogoleri wachiwiri mdziko muno siikuwoneka ntchito yeni yeni yomwe ikugwira
Female
kotero iwo ati mpofunika kuti dziko lino liwunikenso ngati ofesiyi ndiyofunika kapena ayi. A Namiwa anena izi poona kuti ofesi ya mtsogoleri wachiwiriyu kuti igwire ntchito imadalira kupatsidwa mphamvu

komanso chilolezo kuchokera kwa mtsogoleri wa mdziko lino. Iwo anapitilizanso kufotokoza kuti nkofunika kwambili kuti dziko lino liunikire ndikukhazikitsa ndondomeko za ntchito
komanso chilolezo kuchokera kwa mtsogoleri wa mdziko lino. Iwo anapitilizanso kufotokoza kuti nkofunika kwambili kuti dziko lino liunikire ndikukhazikitsa ndondomeko za ntchito
Female
zomwe mtsogoleri wachiwiriyu akuyenera kugwira m’dziko lino. Mwazina, a Namiwa anafotokozanso kuti pakakhala kuti palibe ubale wabwino pakati pa mtsogoleri wadziko ndi wachiwiri wake
zomwe mtsogoleri wachiwiriyu akuyenera kugwira m’dziko lino. Mwazina, a Namiwa anafotokozanso kuti pakakhala kuti palibe ubale wabwino pakati pa mtsogoleri wadziko ndi wachiwiri wake
Female
zimapinga kagwilidwe ka ntchito ka ofesi ya mtsogoleri wachiwiriyu. Pakali pano, ntchito yomwe wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima akugwira siyikudziwika kwenikweni
zimapinga kagwilidwe ka ntchito ka ofesi ya mtsogoleri wachiwiriyu. Pakali pano, ntchito yomwe wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulosi Chilima akugwira siyikudziwika kwenikweni
Female
chifukwa mu chaka cha 2022 mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera adalengeza kuti asiya kupereka ntchito kwa a Chilima
chifukwa mu chaka cha twente twente thu mtsogoleri wa dziko lino a Lazalasi Chakwera adalengeza kuti asiya kupereka ntchito kwa a Chilima
Female
Izi zidachitika chifukwa choti a Chilima akuwaganizira kuti adalandira ziphuphu. Mu chaka cha 2018, a Chilima adasiya kuwapatsa ntchito pomwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino panthawiyo a Peter Mutharika
Izi zidachitika chifukwa choti a Chilima akuwaganizira kuti adalandira ziphuphu. Mu chaka cha tuwente eitini, a Chilima adasiya kuwapatsa ntchito pomwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino panthawiyo a Peter Mutharika
Female
Panthawiyi, a Chilima adalengeza kuti atuluka chipani cholamula cha DPP ndikuyambitsa chawo
Panthawiyi, a Chilima adalengeza kuti atuluka chipani cholamula cha Dipipi ndikuyambitsa chawo
Female
Pomwe anthu ena amadzudzula mkulu wa ku Mulanje yemwe anatengera ku polisi nkhumba yake yomwe imakanika kufa, apolisi ati panalibe vuto kutelo ndipo alimbikitsa anthu kuti adzipita ndi nkhani zawo

za mtundu uli onse adzathandizidwa bwino. Lamulungu lapitali pa 14 January, anthu ochuluka anakhamukira pa polisi ya Mulanje kukaona nkhumba yomwe imakanika kufa
za mtundu uli onse adzathandizidwa bwino. Lamulungu lapitali pa fotini Januwale, anthu ochuluka anakhamukira pa polisi ya Mulanje kukaona nkhumba yomwe imakanika kufa
Female
pomwe a Gresham Thunga omwe anagula nkhumbayi kwa munthu wina, anayimika manja kamba koti analephera kuipha atayesera njira zonse kwa maola oposa asanu, 5
pomwe a Gileshamu Thunga omwe anagula nkhumbayi kwa munthu wina, anayimika manja kamba koti analephera kuipha atayesera njira zonse kwa maola oposa asanu faifi
Female
A Thunga anauza nyumba zofalitsa nkhani mdziko muno kuti iwo agwira ntchito yopha nyama kwa zaka zoposa khumi koma zomwe zinachitika pa tsikuli zinawadabwitsa kwambiri ponena kuti anali asanazionepo

Iwo anati ataopsedwa kuti nkhumbayi siyimafa ngakhale pomwe anaibaya pa khosi komaso kuithira madzi otentha kwambiri, anapanga chiganizo chopita nayo ku polisiko kuti akawaunikire zoyenera kuchita

podziwa kuti nzeru zayekha anaviika nsima m’madzi. Madzulo a tsiku lomweli, munthu yemwe anawagulitsa a Thunga nkhumbayo anakwanitsa kupha chiwetocho
podziwa kuti nzeru zayekha anaviika nsima m’madzi. Madzulo a tsiku lomweli, munthu yemwe anawagulitsa a Thunga nkhumbayo anakwanitsa kupha chiwetocho
Female
Izi zitachitika, anthu ena mdziko muno makamaka m’masamba anchezo, anadzudzula a Thunga pa zomwe anapangazo
Izi zitachitika, anthu ena mdziko muno makamaka m’masamba anchezo, anadzudzula a Thunga pa zomwe anapangazo
Female
ponena kuti zinali zolakwika kwambiri ndipo ena anati uku kunali kuyigwiritsa ntchito polisi molakwika. Koma anthu atayankhula zonsezi, apolisi mdziko muno kudzera pa zomwe ayika pa tsamba lawo la fesibuku

ati palibe cholakwika chilichonse pa zomwe mkuluyu anapanga kutengera nkhumbayo ku polisi ndipo alimbikitsaso anthu ena kuti adzipita ku polisiko ndi nkhani zawo za ntundu uli onse
ati palibe cholakwika chilichonse pa zomwe mkuluyu anapanga kutengera nkhumbayo ku polisi ndipo alimbikitsaso anthu ena kuti adzipita ku polisiko ndi nkhani zawo za ntundu uli onse
Female
Muli ndi ufulu kubwera ndi nkhani zanu ku Police ndipo tizakuthandizani kapena kukuunikirani koyenera kupita nazo, analemba choncho akuluakulu a polisi pa tsamba lawo la fesibuku
Muli ndi ufulu kubwera ndi nkhani zanu ku Police ndipo tizakuthandizani kapena kukuunikirani koyenera kupita nazo, analemba choncho akuluakulu a polisi pa tsamba lawo la fesibuku
Female
pomwe anaika chithuzi chotsindika kuti panalibe vuto kupita ndi nkhumbayo ku polisiko. Pa chithunzi chomwe chinaponyedwa pa tsambali, akuluakulu a Malawi Police Service
pomwe anaika chithuzi chotsindika kuti panalibe vuto kupita ndi nkhumbayo ku polisiko. Pa chithunzi chomwe chinaponyedwa pa tsambali, akuluakulu a Malawi Polisi sevisi
Female
alembapo kuti, Za nkhumba ija zatha bwino Apolisi ndi abale anu, Timathandiza ndi kuunikira mwaukadaulo pa vuto lili lonse lomwe mwakumana nalo.
alembapo kuti, Za nkhumba ija zatha bwino Apolisi ndi abale anu, Timathandiza ndi kuunikira mwaukadaulo pa vuto lili lonse lomwe mwakumana nalo.
Female
Pakadali pano anthu ena akuyamikira Malawi Police Service kamba kothandiza pa nkhani ya nkhumbayi pomwe ena akupitililabe kudzudzula kuti uku ndikutengera ntchito za nthambi yosungutsa chitetezoyi pa mgong’o
Pakadali pano anthu ena akuyamikira Malawi Polisi sevisi kamba kothandiza pa nkhani ya nkhumbayi pomwe ena akupitililabe kudzudzula kuti uku ndikutengera ntchito za nthambi yosungutsa chitetezoyi pa mgong’o
Female
Inu azibambo a COSOMA mukundisala bwanji, Wafunsa Jetu. Jetu walira chokweza pamene bungwe la Copyright Association of Malawi COSOMA
Inu azibambo a KOSOMA mukundisala bwanji, Wafunsa Jetu. Jetu walira chokweza pamene bungwe la Kopelaiti asosiyesgoni ofu Malawi KOSOMA
Female
silidamupatseko yachipuputa misonzi pamene bungweli lapereka makobidi kwa oyimba osiyanasiyana mdziko muno ndipo iye akufunsa kuti a COSOMA akumusala bwanji
silidamupatseko yachipuputa misonzi pamene bungweli lapereka makobidi kwa oyimba osiyanasiyana mdziko muno ndipo iye akufunsa kuti a KOSOMA akumusala bwanji
Female
Jetu wayankhula izi kudzera munkanema yemwe Malawi24 yaona ndipo izi ndi zomwe wafotokoza: Eee ndikufunseni inu azibambo aku COSOMA
Jetu wayankhula izi kudzera munkanema yemwe Malawi twente folo yaona ndipo izi ndi zomwe wafotokoza: Eee ndikufunseni inu azibambo aku KOSOMA
Female
ine ndi Jetu azanga onse mwapatsa 2 miliyoni 2 miliyoni oyimba ine osandipatsa malo mpakananso mwagulira malo
ine ndi Jetu azanga onse mwapatsa Thu miliyoni Thu miliyoni oyimba ine osandipatsa malo mpakananso mwagulira malo
Female
nanga ine mukundisala bwanji, Mundiuze inu a COSOMA ine ndi Jetu. Jetu wayankhula izi kutsatira bungwe la COSOMA litapereka ndalama kwa oyimba osiyanasiyana mdziko muno
nanga ine mukundisala bwanji, Mundiuze inu a KOSOMA ine ndi Jetu. Jetu wayankhula izi kutsatira bungwe la KOSOMA litapereka ndalama kwa oyimba osiyanasiyana mdziko muno
Female
Driemo ndi Eli Njuchi ndi omwe alandira ndalama zokwana 5miliyoni kwacha. Omwe alandira ndalama zokwana 4 miliyoni kwacha ndi oyimba monga Gibo Pearson komanso Skeffa Chimoto
Dilioyemo ndi Eli Njuchi ndi omwe alandira ndalama zokwana faifi miliyoni kwacha. Omwe alandira ndalama zokwana folo miliyoni kwacha ndi oyimba monga Gibo Piyasoni komanso Sikefa Chimoto
Female
Pamene Zeze Kingstone, Namadingo, Janta, Wikise, Lucius Banda ndi Kell Kay alandira ndalama zokwana 3 miliyoni kwacha
Pamene Zeze King’isitoni, Namadingo, Janta, Wikise, Lusiyasi Banda ndi Kelo kei alandira ndalama zokwana fili miliyoni kwacha
Female
PaMndandanda wa ma 2 miliyoni pali oyimba monga Zonke , Great Angels Choir, Malinga, Dan Lu, Azizi, Jay Jay Cee, Rashley, Atoht Manje Pamene pa ndandanda womaliza wa ma 1 miliyoni kwacha
PaMndandanda wa ma Thu miliyoni pali oyimba monga Zonke , Gileti enjelozi kwaya, Malinga, Dani Lu, Azizi, Jeyi Jeyisi , Rashile, Atoti Manje Pamene pa ndandanda womaliza wa ma wani miliyoni kwacha
Female
pali oyimba monga Ace Jizzy, Beejay, Gwamba , Waxy Kay, Guntolah, Henry zar, DNA, Billy Kaunda, Lawi, Mlaka, Suffix, Anthony Makondetsa, Ma Blacks, Avokado, Hilco, Keturah
pali oyimba monga Esijizece Jize, Bijeyi, Gwamba , Wakise keyi, Guntola, Henele za, Dienie, Bile Kaunda, Lawi, Mlaka, Safikisi, Anthone Makondetsa, Ma Blulakisi, Avokado, Hiluko, Ketura
Female
Moses Makawa, Nesnes, Joseph Nkasa, Phyzix, Pop Young , Walycris, Tremour, komanso Lay B Salima
Mozesi Makawa, Nesinesi, Josefe Nkasa, Fizikisi, Popu Yang’i , Walekhilisi, Thilema, komanso Leyi Bi Salima
Female
Sukulu ya ukachenjede ya Luanar yapereka zilango kwa ophunzira okwana 19 kamba kopezeka olakwa pa mlandu owonera mayeso ndipo atatu mwa ophunzirawa awachotsa sukulu
Sukulu ya ukachenjede ya Luwana yapereka zilango kwa ophunzira okwana Naintini kamba kopezeka olakwa pa mlandu owonera mayeso ndipo atatu mwa ophunzirawa awachotsa sukulu
Female
Ophunzira pamene khumi ndi anayi ayimitsidwa sukulu kwa zaka ziwili, ena chaka chimodzi pamene awili alandira chenjezo
Ophunzira pamene khumi ndi anayi ayimitsidwa sukulu kwa zaka ziwili, ena chaka chimodzi pamene awili alandira chenjezo
Female
Malingana ndi kalata yomwe sukuluyi yatulutsa, ophunzirawa alandira zilangozi kamba kopezeka ndi lamya za m’manja mchipinda cholembera mayeso
Malingana ndi kalata yomwe sukuluyi yatulutsa, ophunzirawa alandira zilangozi kamba kopezeka ndi lamya za m’manja mchipinda cholembera mayeso
Female
kupezeka ndima likasa, kusinthana notsi, komanso kulemba mayeso popanda kulembetsa. Mmasiku apitawo, sukulu ya ukachenjede ya Malawi Business of Applied Science (MUBAS)
kupezeka ndima likasa, kusinthana notsi, komanso kulemba mayeso popanda kulembetsa. Mmasiku apitawo, sukulu ya ukachenjede ya Malawi Bizinesi ofu apulayidi sayansezi (MUBASI)
Female
idachotsanso ophunzira ena kamba kowonera mayeso ndipo nayonso University of Malawi (UNIMA) idalengezanso kuti yapereka zilango kwa ophunzira ochita mchitidwewu
idachotsanso ophunzira ena kamba kowonera mayeso ndipo nayonso Yumivesite ofu Malawi (YUNIMA) idalengezanso kuti yapereka zilango kwa ophunzira ochita mchitidwewu
Female
Vuto lakuonera mayeso likukura msukulu za ukachenjedezi kamba koti ambili amatangwanika ndi zisangalalo mmalo mopeza nthawi yomawerenga ndipo pamapeto pake amapeza kuti kuonera ndiyo njira yabwino

Mboni zambali ya Boma zatsiliza kuperekera umboni pamulandu wa a Bon Kalindo. Mboni zisanu zambali ya Boma zatsiliza kuperekera umboni pamulandu wamkulu wa Bungwe la Malawi First a Bon Kalindo
Mboni zambali ya Boma zatsiliza kuperekera umboni pamulandu wa a Boni Kalindo. Mboni zisanu zambali ya Boma zatsiliza kuperekera umboni pamulandu wamkulu wa Bungwe la Malawi Fesiti a Boni Kalindo
Female
omwe akuwayimba mulandu owaganizira kuti adayambitsa zipolowe potsatira ziwonetsero zomwe adachititsa pa 23 November mu mzinda wa Zomba
omwe akuwayimba mulandu owaganizira kuti adayambitsa zipolowe potsatira ziwonetsero zomwe adachititsa pa Twente fili Novemba mzinda wa Zomba
Female
Zina mwambonizo ndi apolisi anayi omwe ndi Stella Likukuta, Harry Dongolosi, Inspector Gauti, komanso Assistant Superintendent Isaac Mdala
Zina mwambonizo ndi apolisi anayi omwe ndi Sitela Likukuta, Hare Dongolosi, Insipekita Gauti, komanso Asisitanti supulitendanti Aizeki Mdala
Female
Onsewa ndi ofudzufuza milandu ya upandu ku nthammbi ya a Police ndipo winanso yemwe waperekera nawo umboni pankhani yomweyi
Onsewa ndi ofudzufuza milandu ya upandu ku nthammbi ya a Polisi ndipo winanso yemwe waperekera nawo umboni pankhani yomweyi
Female
ndiyemwe amagwira ntchito kumalo ogulitsira zokumwa a Kangaroo ku Chinamwali Township a Christopher Ndanga
ndiyemwe amagwira ntchito kumalo ogulitsira zokumwa a Kangaluu ku Chinamwali Taunishipi a Khilisitofa Ndanga
Female
A Ndanga adauza bwalo kuti tsiku lomwe kudachitika ziwonetsero anthu ena omwe sakudziwika adabwera masana cha m’ma 2 koloko kudzaba zokumwa zomwe ndi zandalama pafupi fupi 8.5 million kwacha
A Ndanga adauza bwalo kuti tsiku lomwe kudachitika ziwonetsero anthu ena omwe sakudziwika adabwera masana cha m’ma thu koloko kudzaba zokumwa zomwe ndi zandalama pafupi fupi eiti pointi faifi million kwacha
Female
Poyankhula ndi Malawi24, Loya yemwe akuyimira a Bon Kalindo pamulanduwu a Timothy Chirwa adati gawo loyamba lamulanduwu latha akungodikilira bwalo kuti liwunikire zonse zomwe mboni zapereka
Poyankhula ndi Malawi twente folo, Loya yemwe akuyimira a Boni Kalindo pamulanduwu a Timofe Chirwa adati gawo loyamba lamulanduwu latha akungodikilira bwalo kuti liwunikire zonse zomwe mboni zapereka
Female
ndipo lidzagamule ngati a Bon Kalindo alindi mulandu okuti ayankhe kapena ayi pa 21 February
ndipo lidzagamule ngati a Boni Kalindo alindi mulandu okuti ayankhe kapena ayi pa twente wani Febuluwale
Female
Yemwe akuyimira Boma pamulanduwu Superintendent Josephine Chigawa adati ndiwokhutira ndi momwe mboni zawo zaperekera umboni
Yemwe akuyimira Boma pamulanduwu Supulitendanti Josefina Chigawa adati ndiwokhutira ndi momwe mboni zawo zaperekera umboni
Female
Yemwe akudzenga mulanduwu Principal Resident Magistrate Martin Chipofya wayamba wayimitsa mulanduwu mpaka pa 21 February 2 koloko masana
Yemwe akudzenga mulanduwu Pulinsipo lezidenti majesitileti matini Chipofya wayamba wayimitsa mulanduwu mpaka pa twente wani febuluwale thu koloko masana
Female
kuti adzagamule ngati kuti a Kalindo alindi mulandu okuti ayankhe kapena ayi. Pamenepa Principal Resident Magistrate Chipofya
kuti adzagamule ngati kuti a Kalindo alindi mulandu okuti ayankhe kapena ayi. Pamenepa Pulinsipo lezidenti majesitileti Chipofya
Female
waudza oyimira Boma pamulanduwu kuti apereke ma submission awo pokutha kwa masiku asanu ndi awiri (7)
waudza oyimira Boma pamulanduwu kuti apereke ma submission awo pokutha kwa masiku asanu ndi awiri (seveni)
Female
kwa omwe akuyimira a Bon Kalindo komanso waudza omwe akuyimira a Kalindo kuti akhale atapereka ma submission awo kumbali yomwe ikuyimira Boma pofika pa 14 February mwezi wa mawa
kwa omwe akuyimira a Bon Kalindo komanso waudza omwe akuyimira a Kalindo kuti akhale atapereka ma submission awo kumbali yomwe ikuyimira Boma pofika pa fotini Febuluwale mwezi wa mawa
Female
Wapampando wa bhodi ya Mulhako wa Alhomwe watsutsa mphekesera yoti bhodiyi yachotsa mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ngati woyang’anira bungweli
Wapampando wa bodi ya Mulakho wa Alomwe watsutsa mphekesera yoti bodiyi yachotsa mtsogoleri wakale wa dziko lino a Pita Mutharika ngati woyang’anira bungweli
Female
Mukuyankhula kwawo pa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Blantyre lachiwiri, Muchanakwaye Mpuluka yemwe ndi wapampando wa bhodiyi
Mukuyankhula kwawo pa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Bulantaya lachiwiri, Muchanakwaye Mpuluka yemwe ndi wapampando wa bodiyi
Female
anati dongosolo ndi mphamvu zochotsa komaso kubwezeretsa amdindo mu bungweli zili ndi bhodi yaikulu imene imasankha komitiyi yosankha kapena kuchotsa amdindo
anati dongosolo ndi mphamvu zochotsa komaso kubwezeretsa amdindo mu bungweli zili ndi bodi yaikulu imene imasankha komitiyi yosankha kapena kuchotsa amdindo
Female
Mpuluka wati ndi zabodza zimene nyumba zina zoulutsa mau zikulengeza kuti bungweli lachotsa a Munthalika pa udindowu
Mpuluka wati ndi zabodza zimene nyumba zina zoulutsa mau zikulengeza kuti bungweli lachotsa a Munthalika pa udindowu
Female
Bungwe lathu limalemekeza maganizo a aliyese. Mphamvu zopanga chiganizo sizikhala kwa munthu m’modzi ndipo izi zikapitirira tikasuma Ku bwalo la milandu, atero a Mpuluka
Bungwe lathu limalemekeza maganizo a aliyese. Mphamvu zopanga chiganizo sizikhala kwa munthu m’modzi ndipo izi zikapitirira tikasuma Ku bwalo la milandu, atero a Mpuluka
Female