audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Bushiri wati ndege yomwe akulingalira kugulayo, ndiyoti izinyamula anthu omwe amabwera mdzikomuno kuchokera maiko akunja kudzkhalanawo pa mapemphero osiyanasiyana.
Bushiri wati ndege yomwe akulingalira kugulayo, ndiyoti izinyamula anthu omwe amabwera mdzikomuno kuchokera maiko akunja kudzkhalanawo pa mapemphero osiyanasiyana.
female
Omwe iye amapangitsa makamaka mu m’zinda wa Lilongwe. Ndiri ndi malingaliro ofuna kugula ndege yoti izinyamula anthu kubwera nawo ku mapemphero athu. Tikulemeretsa company za ndege.
Omwe iye amapangitsa makamaka mu m’zinda wa Lilongwe. Ndiri ndi malingaliro ofuna kugula ndege yoti izinyamula anthu kubwera nawo ku mapemphero athu. Tikulemeretsa kampani za ndege.
female
Watero Bushiri mu uthenga womwe wawulemba mchingerezi pa tsamba lake la Facebook. Anthu ambiri omwe akhamukira ku tsambali kukayikira ndemanga, ayamikira mneneriyu kamba ka maganizowa.
Watero Bushiri mu uthenga womwe wawulemba mchingerezi pa tsamba lake la Fesibuku. Anthu ambiri omwe akhamukira ku tsambali kukayikira ndemanga, ayamikira mneneriyu kamba ka maganizowa.
female
Ponena kuti izi zithanso kuthandiza kupititsa patsogolo ntchito zokopa alendo mdzikomuno, pamapeto pake nkumapititsaso chuma cha dzikolino patsogolo.
Ponena kuti izi zithanso kuthandiza kupititsa patsogolo ntchito zokopa alendo mdzikomuno, pamapeto pake nkumapititsaso chuma cha dzikolino patsogolo.
female
Chithawireni mdziko la South Africa mchaka cha 2020, komwe akuti kunali chiopsezo choti akanatha kuphedwa, Bushiri wakhala m’modzi mwa anthu,komanso zinthu zomwe zapangitsa kuti dzikolino.
Chithawireni mdziko la Sowufi Afirika mchaka cha tuwente tuwente, komwe akuti kunali chiopsezo choti akanatha kuphedwa, Bushiri wakhala m’modzi mwa anthu,komanso zinthu zomwe zapangitsa kuti dzikolino.
female
Lizilandira alendo ochuluka kuchokera m’maiko ena. Ma passport akukanika kutuluka ku Immigration, mavuto akuoneka kuti sakutha ku nthambbi yowona za anthu olowa ndi kutuluka mdzikomuno. Immigration.
Lizilandira alendo ochuluka kuchokera m’maiko ena. Ma pasipoti akukanika kutuluka ku Imigireshoni, mavuto akuoneka kuti sakutha ku nthambbi yowona za anthu olowa ndi kutuluka mdzikomuno, Imigireshoni.
female
Pomwe nthambiyi yati ikukanika kutulutsa ziphaso zoyendera, ma passport. Izi ndi malingana ndi uthenga wa nthambiyi kupita kwa Malawi. Tikudziwitsani a Malawi kuti makina athu otulutsira ziphaso zoyendera passport,
Pomwe nthambiyi yati ikukanika kutulutsa ziphaso zoyendera, mapasipoti. Izi ndi malingana ndi uthenga wa nthambiyi kupita kwa Malawi. Tikudziwitsani a Malawi kuti makina athu otulutsira ziphaso zoyendera pasipoti,
female
Ali ndi vuto ndipo pakadalipano, sitikutulutsa ziphasozi, koma anthu athu okonza ali nkati mokonza makinawa, ndipo zikatheka tikudziwitsani.
Ali ndi vuto ndipo pakadalipano, sitikutulutsa ziphasozi, koma anthu athu okonza ali nkati mokonza makinawa,ndipo zikatheka tikudziwitsani.
female
Yatero mbali ya uthengawo. Nthambiyi yakhala ikukumana ndi mavuto ena pomwe nthambiyi, inadzayimitsapo kutulutsa ziphaso, ponena kuti imakoza kaye ndondomeko zatsopano.
Yatero mbali ya uthengawo. Nthambiyi yakhala ikukumana ndi mavuto ena pomwe nthambiyi, inadzayimitsapo kutulutsa ziphaso, ponena kuti imakoza kaye ndondomeko zatsopano.
female
Chithetsereni contract ndi company yomwe imasindikiza passport mu nthambiyi, nthambiyi yakhala ikukumana ndi zovuta zambiri pomwe anthu akahala akudandawula kuti nthambiyi ikumachedwa kutulutsa ma passport.
Chithetsereni kontirakiti ndi kampani yomwe imasindikiza pasipoti mu nthambiyi, nthambiyi yakhala ikukumana ndi zovuta zambiri pomwe anthu akahala akudandawula kuti nthambiyi ikumachedwa kutulutsa ma pasipoti.
female
Mwachitsazo passport ya 90,000 kwacha, ikuyenera kuti masiku khumi, 10, ikhale itatuluka pomwe passport ya 180,000 kwacha ikuyenera kuti izituluka m’masiku atatu.
Mwachitsazo pasipoti ya Nayinte sauzandi kwacha, ikuyenera kuti masiku khumi, teni, ikhale itatuluka pomwe pasipoti ya wani handiredi andi eyite sauzandi kwacha ikuyenera kuti izituluka m’masiku atatu.
female
Koma izi sizikumakhala choncho. Mtsogoleri wa team ya Mighty Mukuru Wanderers, Thom Mpinganjira, wachenjeza wochemerera team yi, makamaka aku Lilongwe pankhani yoyambitsa ziwawa.
Koma izi sizikumakhala choncho. Mtsogoleri wa timu ya Mayite Mukuru Wandarazi, Thomu Mpinganjira, wachenjeza wochemerera timuyi, makamaka aku Lilongwe pankhani yoyambitsa ziwawa.
female
Ndipo wati masewero aliwonse aziyitanitsa a police wokhala ndi mfuti kuti athane ndi maliwongo aliyense. Izi ndi malingana ndi kanema wina yemwe anthu akugawana pa masamba a nchezo.
Ndipo wati masewero aliwonse aziyitanitsa a polisi wokhala ndi mfuti kuti athane ndi maliwongo aliyense. Izi ndi malingana ndi kanema wina yemwe anthu akugawana pa masamba a nchezo.
female
Yemwe akuwonetsa mpondamatikiyu akuyankhula za team yawo ya wanderers pankhani ya ziwawa zomwe wochemerera team yovala makaka a blue yi anachita ku masewero ena chakachatha.
Yemwe akuwonetsa mpondamatikiyu akuyankhula za timu yawo ya wandarazi pankhani ya ziwawa zomwe wochemerera timu yovala makaka a buluyi anachita ku masewero ena chakachatha.
female
Mtsogoleri wa teamyi, wati ndi wokhumudwa komaso watopa ndi zindapusa zomwe team ya wanderers yakhala ikulandira kamba ka mchitidwe wa zipolowe pa masewera ena angapo.
Mtsogoleri wa timuyi, wati ndi wokhumudwa komaso watopa ndi zindapusa zomwe timu ya wandarazi yakhala ikulandira kamba ka mchitidwe wa zipolowe pa masewera ena angapo.
female
Ndipo wati tsopano wapeza njira zingapo zomwe akuti zithandiza mchitidwewu kutheratu. Mwazina a Mpinganjira ati pamasewero aliwonse omwe NOMA izisewera chaka chino.
Ndipo wati tsopano wapeza njira zingapo zomwe akuti zithandiza mchitidwewu kutheratu. Mwazina a Mpinganjira ati pamasewero aliwonse omwe NOMA izisewera chaka chino.
female
Makamaka omwe aziseweredwera mu mzinda wa Lilongwe, Iye ngati nkulu wa team, aziyitanitsa a police okhala ndi mfuti kuti azikakhazikitsa bata, komanso kuthana ndi aliyense wofuna kuyambitsa chipwirikiti.
Makamaka omwe aziseweredwera mu mzinda wa Lilongwe, Iye ngati nkulu wa timu, aziyitanitsa a polisi okhala ndi mfuti kuti azikakhazikitsa bata, komanso kuthana ndi aliyense wofuna kuyambitsa chipwirikiti.
female
Ku Lilongwe muwawuze, ndizipanga hayala apolice a mfuti aja, osati aja amanyamula ndodo ayi. Muwauze ma supporter a Wanderers ku Lilongwe, akangopezekanso, kukupita PMF.
Ku Lilongwe muwawuze, ndizipanga hayala apolisi a mfuti aja, osati aja amanyamula ndodo ayi. Muwauze masapota a Wandarazi ku Lilongwe, akangopezekanso, kukupita PI EMU EFU.
female
Game iliyonse ya Wanderers ku Lilongwe, ndizipanga hayala PMF ngati sakusamala. Wakalipa Mpinganjira.
Gemu iliyonse ya Wandarazi ku Lilongwe, ndizipanga hayala PI EMU EFU ngati sakusamala. Wakalipa Mpinganjira.
female
Izi zikuchitika pomwe mkuluyi wathetsa ma committee angapo, a team ya Wanderers, pomwe akuchita chothekera kuti NOMA iyambirenso kumwa wa mkaka, potsatira kulephera kutenga chikho chilichonse mchaka cha 2023.
Izi zikuchitika pomwe mkuluyi wathetsa makomiti angapo, a timu ya Wandarazi, pomwe akuchita chothekera kuti NOMA iyambirenso kumwa wa mkaka, potsatira kulephera kutenga chikho chilichonse mchaka cha tuwente tuwente-firi.
female
Chaka chatha team yi, inalipitsidwa chindapusa cha 22,000,000 kwacha, potsatira chipwirikiti chomwe chinachitika pa masewera ake ndi Silver strikers.
Chaka chatha timuyi, inalipitsidwa chindapusa cha tuwente-thu miliyoni kwacha, potsatira chipwirikiti chomwe chinachitika pa masewera ake ndi Siliva sitirayikazi.
female
Pomwe wochemerera team yi, anawononga wina mwa katundu pa bwalo la masewero la Bingu ku Lilongwe, kamba kosakondwa ndi chiganizo cha woyimbira Godfrey Nkhakananga.
Pomwe wochemerera timuyi, anawononga wina mwa katundu pa bwalo la masewero la Bingu ku Lilongwe, kamba kosakondwa ndi chiganizo cha woyimbira Godifure Nkhakananga.
female
Kupatula apo team yi inalipitsidwanso chindapusa china kamba kolephera kusewera masewero a chibwereza ndi Silver strikers mu mpikisano wa Airtel Top 8.
Kupatula apo timu yi inalipitsidwanso chindapusa china kamba kolephera kusewera masewero a chibwereza ndi Siliva sitirayikazi mu mpikisano wa Eyatelo Topu eyiti.
female
Komanso inapatsidwa chilango, choti isatengensonawo gawo mu mpikisano uliwonse wokonzedwa ndi bungwe la FAM, koma mwa mwayi, team yi inakhululukidwa.
Komanso inapatsidwa chilango, choti isatengensonawo gawo mu mpikisano uliwonse wokonzedwa ndi bungwe la FAMU, koma mwa mwayi, timuyi inakhululukidwa.
female
Magetsi avuta pa chipatala cha Mzimba. Chipatala cha Mzimba, chikumagwiritsa ntchito ndalama zosachepera 800,000 kwacha pa tsiku kugula mafuta a generator.
Magetsi avuta pa chipatala cha Mzimba. Chipatala cha Mzimba, chikumagwiritsa ntchito ndalama zosachepera eyiti handiredi sauzandi kwacha pa tsiku kugula mafuta a jenereta.
female
Kamba ka vuto la kuthimathima kwa magetsi pa chipatalachi. Malawi 24, yapeza kuti chipatala cha chikulu cha boma la Mzimba, chikumagula ma litre apakati 250 ndi 300 pa tsiku oyatsira generator.
Kamba ka vuto la kuthimathima kwa magetsi pa chipatalachi. Malawi tuwnte-folo, yapeza kuti chipatala cha chikulu cha boma la Mzimba, chikumagula malita apakati thu handiredi and fifite ndi firi handiredi pa tsiku oyatsira jenereta.
female
Mwachitsanzo, pakati pa 30 December, 2023 mpaka pa 01 January, 2024, Chipatalachi chinagwiritsa ntchito ndalama zoposera 2,460,600,000 kwacha.
Mwachitsanzo, pakati pa sete Disemba, tuwente tuwente-firi mpaka pa wani, Januware, tuwente tuwente-folo, Chipatalachi chinagwiritsa ntchito ndalama zoposera thu miliyoni, folo handiredi andi sikisite sikisi handiredi kwacha.
female
Pogula mafuta a generator, pomwe anthu anakhala mawola 72, opanda magetsi a ESCOM. Francis Liyati yemwe amayankhulapo pa zinthu zosiyanasiyana zochitika mdzikomuno.
Pogula mafuta a jeneretar, pomwe anthu anakhala mawola 72, opanda magetsi a ESIKOMU. Furansisi Liyati yemwe amayankhulapo pa zinthu zosiyanasiyana zochitika mdzikomuno.
female
Wati ndizodabwitsa kuti pomwe boma linalengeza kuti magetsi asiya kuvuta, anthu m’boma la Mzimba, akuvutikabe.
Wati ndizodabwitsa kuti pomwe boma linalengeza kuti magetsi asiya kuvuta, anthu m’boma la Mzimba, akuvutikabe.
female
Ndizovetsa chisoni kwambiri kuti ndalama za nkhaninkhani, zomwe zikupita kogula mafuta kamba ka vuto la magetsi, zikanagwira ntchito ina.
Ndizovetsa chisoni kwambiri kuti ndalama za nkhaninkhani ,zomwe zikupita kogula mafuta kamba ka vuto la magetsi, zikanagwira ntchito ina.
female
Ndikuwona ngati unduna wazamagetsi komanso phungu waderali yemwenso ali a nduna a Jacob Hara, alowererepo, chifukwa zikuwonetsa kuti vuto la magetsi ku Mzimba lafika povuta kwambiri. Anatero a Liyati.
Ndikuwona ngati unduna wazamagetsi komanso phungu waderali yemwenso ali a nduna a Jakobo Hara, alowererepo, chifukwa zikuwonetsa kuti vuto la magetsi ku Mzimba lafika povuta kwambiri. Anatero a Liyati.
female
Posachedwapa a mabungwe omwe asali a boma ku Mzimba, motsogozedwa ndi wapampando wawo Christopher Merere, anapita ku office ya ESCOM m’bomali.
Posachedwapa a mabungwe omwe asali a boma ku Mzimba, motsogozedwa ndi wapampando wawo Khirisitofa Merere, anapita ku ofesi ya ESIKOMU m’bomali.
female
Ndikuchita zokambirana kuti amve vuto la magetsi lomwe tsopano lasanduka chipsinjo. Koma omwe akungogwirizira udindo woyang’anira office ya Mzimba ya ESCOM, a Cuthbert Ngwira ndi azawo.
Ndikuchita zokambirana kuti amve vuto la magetsi lomwe tsopano lasanduka chipsinjo. Koma omwe akungogwirizira udindo woyang’anira ofesi ya Mzimba ya ESIKOMU, a Kafibeti Ngwira ndi azawo.
female
Anakanika kuyankha mafunso omwe amabungwewa anafunsa, ponena kuti iwo sali wololedwa kuyankhula chilichonse. A Merere awuza Malawi 24, kuti lolemba pa 8, January, 2024.
Anakanika kuyankha mafunso omwe amabungwewa anafunsa, ponena kuti iwo sali wololedwa kuyankhula chilichonse. A Merere awuza Malawi tuwnte-folo, kuti lolemba pa eyiti Januware, tuwente tuwente-folo.
female
Nthawi 10 koloko m’mawa, akhala akuchita mkumano ndi akuluakulu a ESCOM ochokera ku office yayikulu yachigawo cha kumpoto.
Nthawi teni koloko m’mawa, akhala akuchita mkumano ndi akuluakulu a ESIKOMU ochokera ku ofesi yayikulu yachigawo cha kumpoto.
female
Naye mkula wa ESCOM, ku chigawo cha kumpoto Thomas Nzumara, anatsimikiza kuti akhala akukumana ndi amabungwewo kuti awafotokozere ngati pali vuto.
Naye mkula wa ESIKOMU, ku chigawo cha kumpoto Thomasi Nzumara, anatsimikiza kuti akhala akukumana ndi amabungwewo kuti awafotokozere ngati pali vuto.
female
Anthu ena wokhudzidwa m’bomali, akuganiza kuti kuzimazima kwa magetsi komwe kukuchitikaku, kwadza kamba ka wogwira ntchito ena omwe akufuna kunyazitsa boma komansso kudzetsa udani pakati pa anthu ndi bomalawo.
Anthu ena wokhudzidwa m’bomali, akuganiza kuti kuzimazima kwa magetsi komwe kukuchitikaku, kwadza kamba ka wogwira ntchito ena omwe akufuna kunyazitsa boma komanso kudzetsa udani pakati pa anthu ndi bomalawo.
female
DODMA, yalangiza maanja omwe akulandira chakudya, kuti alimbikire ntchito zawo za tsiku ndi tsiku. Nthambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzidzi mdzikomuno ya DODMA.
DODIMA, lalangiza maanja omwe akulandira chakudya, kuti alimbikire ntchito zawo za tsiku ndi tsiku. Nthambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzidzi mdzikomuno ya DODIMA.
female
Yalangiza maanja amene akulandira chakudya kuchokera kuboma kudzera ku nthambiyi kuti apitirize kugwira ntchito zawo za tsiku ndi tsiku, kuti akhale odzidalira pawokha.
Yalangiza maanja amene akulandira chakudya kuchokera kuboma kudzera ku nthambiyi kuti apitirize kugwira ntchito zawo za tsiku ndi tsiku, kuti akhale odzidalira pawokha.
female
Wanena izi ndi mulembi wankulu ku nthambiyi, a Charles Kalemba m’maboma a Karonga ndi Chitipa, komwe amakhazikitsa ntchito yothandiza maanja omwe akusowa chakudya.
Wanena izi ndi mulembi wankulu ku nthambiyi, a tchalosi Kalemba m’maboma a Karonga ndi Chitipa, komwe amakhazikitsa ntchito yothandiza maanja omwe akusowa chakudya.
female
Kalemba wati, anthuwa adzikhuthule kwa thunthu, kugwira ntchito m’minda ndi m’madimba, osati manja lende. Ngati boma tikuzindikira kuti tinakhudzidwa ndi ng’amba yoopsa chakachatha.
Kalemba wati, anthuwa adzikhuthule kwa thunthu, kugwira ntchito m’minda ndi m’madimba, osati manja lende. Ngati boma tikuzindikira kuti tinakhudzidwa ndi ng’amba yoopsa chakachatha.
female
Nduna yowona za ngozi yogwa mwadzidzidzi, mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera, anabwera kudzakuyenderani, tikudziwa kuti wanjala sangalowe m’munda. Pomwe mwadya musakhale tambalale.
Nduna yowona za ngozi yogwa mwadzidzidzi, mtsogoleri wadziko lino a Lazarasi Chakwera, anabwera kudzakuyenderani, tikudziwa kuti wanjala sangalowe m’munda. Pomwe mwadya musakhale tambalale.
female
Limbikirani ntchito kuti inu ndi dzikolonse, likhale lodzidalira. Ndizovetsa chisoni kuti ngati dziko tikupitirira kumavutika ndi njala, pomwe tili ndi nyanja ndi mitsinje yochuluka.
Limbikirani ntchito kuti inu ndi dzikolonse, likhale lodzidalira. Ndizovetsa chisoni kuti ngati dziko tikupitirira kumavutika ndi njala, pomwe tili ndi nyanja ndi mitsinje yochuluka.
female
Anatero a Kalemba. Ndipo m’mawu awo, mfumu yayikulu Kiripula ya m’boma la Karonga anati bomali ndilodalitsika ndi madzi ndipo ulimi wathirira ndiwotheka, zikungofunika kuti anthu ayikepo chidwi.
Anatero a Kalemba. Ndipo m’mawu awo, mfumu yayikulu Kiripula ya m’boma la Karonga anati bomali ndilodalitsika ndi madzi ndipo ulimi wathirira ndiwotheka, zikungofunika kuti anthu ayikepo chidwi.
female
Maanja 18,000, ndiwomwe apindule ku Karonga ndipo m’boma la Chitipa ,maanja 5778,ndiwomwe alandire thandinzo pansi pa ndondomekoyi.
Maanja eyitini sauzandi, ndiwomwe apindule ku Karonga ndipo m’boma la Chitipa, maanja fayifi sauzandi seveni handiredi andi sevente-eyiti, ndiwomwe alandire thandinzo pansi pa ndondomekoyi.
female
Ntchitoyi ikuchitika pansi pa ndondomeko ya chaka cha 2023-2024, lean season response, yomwe ikufikira anthu oposa 4.4.000,000, m’maboma onse 28 komaso m‘mizinda inayi ya mdziko lino.
Ntchitoyi ikuchitika pansi pa ndondomeko ya chaka cha tuwente tuwente-firi - tuwente tuwente-folo, lini sozoni risiponsi, yomwe ikufikira anthu oposa folo poyinti folo miliyoni, m’maboma onse tuwente-eyiti komaso m‘mizinda inayi ya mdziko lino.
female
Kuli kusambwadzana za mkabudula uku, pomwe mtsutso wa ubwino wokhala ndi degree kapena kungokhala ndi Chilembwe basi, wafika pa mwana wakana phala pakati pa woyimba Dan Lu ndi Cabo Lombwe.
Kuli kusambwadzana za mkabudula uku, pomwe mtsutso wa ubwino wokhala ndi digiri kapena kungokhala ndi Chilembwe basi, wafika pa mwana wakana phala pakati pa woyimba Dani Lu ndi kabo Lombwe.
female
Ndipo nkhaniyi yatsikira ku ma area. Nkhaniyi inayamba pa 19 January, 2024, pomwe woyimba Dan Lufan, analemba patsamba lake la Facebook.
Ndipo nkhaniyi yatsikira ku ma eriya. Nkhaniyi inayamba pa nayintini Januware, tuwente tuwente-folo, pomwe woyimba Dani Lufani, analemba patsamba lake la Fesibuku.
female
Kuyitaniza anthu omutsata omwe iye amati ngakhale kuti alibe tsamba la degree, ndipo lilime lawo silinatambasuke kuti azilankhula chizungu chothyakuka bwino, akukhala moyo wosangalala.
Kuyitaniza anthu omutsata omwe iye amati ngakhale kuti alibe tsamba la digiri, ndipo lilime lawo silinatambasuke kuti azilankhula chizungu chothyakuka bwino, akukhala moyo wosangalala.
female
Onse amene timanenedwa kuti ndife ma survage mafana osatha kuyankhula English, koma timakhala moyo owaposa ama degreewo, bwerani pano mafana aziwindi, 2024 mutiva zigege.
Onse amene timanenedwa kuti ndife ma saveji, mafana osatha kuyankhula ingilishi, koma timakhala moyo owaposa ama digiriwo, bwerani pano mafana aziwindi, tuwente tuwente-folo mutiva zigege.
female
Anatero Dan Lu pa tsamba lake la facebook. Nkaniyi inaveka monyung’unya kwa anthu angapo omwe amathandiza woyimba Cabo Lombwe yemwe naye analemba patsamba lake la facebook.
Anatero Dan Lu pa tsamba lake la fesibuku. Nkaniyi inaveka monyung’unya kwa anthu angapo omwe amathandiza woyimba kabo Lombwe yemwe naye analemba patsamba lake la fesibuku.
female
Ndikutsutsana ndi zomwe Dan Lu analankhulazo, ponena kuti degree ndiyofunika kwambiri pa moyo wa munthu. Lombwe yemwe pano amathandizira woyimba wotchuka Nepman.
Ndikutsutsana ndi zomwe Dani Lu analankhulazo, ponena kuti digiri ndiyofunika kwambiri pa moyo wa munthu. Lombwe yemwe pano amathandizira woyimba wotchuka Nepumani.
female
Wati ndizomvetsa chisoni, kuti Dan Lu azikayankhula mosimbwa pankhani ya degree, pomwe woyimbayu thupi lake likachita honya, amapita kuchipatala komwe amakathandizidwa ndi akatswiri a ma degree akuwanenawo.
Wati ndizomvetsa chisoni, kuti Dani Lu azikayankhula mosimbwa pankhani ya digiri, pomwe woyimbayu thupi lake likachita honya, amapita kuchipatala komwe amakathandizidwa ndi akatswiri a ma digiri akuwanenawo.
female
Zimakhala zomvetsa chisoni ukamamva munthu wankulu akuti degree ndiyopanda ntchito simply because zake zimatheka opanda degree, chosecho akadwala, amathamangira kuchipatala kuti akathandizidwe ndi munthu wa degree.
Zimakhala zomvetsa chisoni ukamamva munthu wankulu akuti digiri ndiyopanda ntchito simpule bikozi zake zimatheka opanda digiri, chosecho akadwala, amathamangira kuchipatala kuti akathandizidwe ndi munthu wa digiri.
female
Ati degree is just a paper, mukadwala osamapita kwa sing’anga bwanji? Anayankha Lombwe pa tsambalake la facebook, chimkulirano chafika posawuzana tsopano, ndipo awiriwa afika polozana zala, kutchulana za mkabudula.
Ati digiri izi jasit e pepa, mukadwala osamapita kwa sing’anga bwanji? Anayankha Lombwe pa tsamba lake la fesibuku, chimkulirano chafika posawuzana tsopano, ndipo awiriwa afika polozana zala, kutchulana za mkabudula.
female
Mpaka Lombwe wafika pomuyalutsa Lufani kuti mwanawake woyamba uja siwake, ndipo akuti woyimbayu, Kalulu anamudutsa m’mphechepeche.
Mpaka Lombwe wafika pomuyalutsa Lufani kuti mwanawake woyamba uja siwake, ndipo akuti woyimbayu, Kalulu anamudutsa m’mphechepeche.
female
Awuzeni anthu chilungamo, munatenga mkazi wa promoter wankulu ku USA, atabwera kudzakupangani sign, nkumusandutsa mkaziwanu.
Awuzeni anthu chilungamo, munatenga mkazi wa puromota wankulu ku YU ESIE, atabwera kudzakupangani sayini, nkumusandutsa mkaziwanu.
female
Awuzeni anthu kuti mwa banidwa pano simungapitenso ku America for 10 years, cause munalandira ma 5 000,000 kwa anthu kuti mupite nawo ku America ngati a band yanu asali oyimba.
Awuzeni anthu kuti mwa banidwa pano simungapitenso ku Amerika fo teni yiyezi, kozi munalandira ma fayifi miliyoni kwa anthu kuti mupite nawo ku Amerika ngati a bandi yanu asali oyimba.
female
Awuzeni anthu kuti mwanawanu uja bambo ake ndi azanu aja, inu simabereka, mawa mupangeso live ina, don't try me, ndakupirirani ndatopa, ndikupatsani zomwe mukufuna.
Awuzeni anthu kuti mwanawanu uja bambo ake ndi azanu aja, inu simabereka. Mawa mupangenso layivi ina, donti thiraye mi, ndakupirirani ndatopa, ndikupatsani zomwe mukufuna.
female
Wateronso Lombwe mu uthenga womwe pakadali pano wawufufuta pa tsamba lake la facebook. Lombwe asanalembe izi patsambalake, Dan Lu anachititsa mkomano wa anthu omutsatira pa tsamba lake la facebook.
Wateronso Lombwe mu uthenga womwe pakadali pano wawufufuta pa tsamba lake la fesibuku. Lombwe asanalembe izi patsamba lake, Dani Lu anachititsa mkomano wa anthu omutsatira pa tsamba lake la fesibuku.
female
Komwe anafotokoza zambiri zazomwe amkatanthawuza pazomwe analemba patsamba lake zokhudza kukhala ndi degree kapena ayi. Iye wati uthenga analembawu, sunali ofuna kunyoza aliyense.
Komwe anafotokoza zambiri zazomwe amkatanthawuza pazomwe analemba patsamba lake zokhudza kukhala ndi digiri kapena ayi. Iye wati uthenga analembawu, sunali ofuna kunyoza aliyense.
female
Ndipo akuti sanaganizire kuti anthu ena ngati Lombwe, atha kudzambatuka, ndikuyamba kumugenda miyala pa zomwe analembazo.
Ndipo akuti sanaganizire kuti anthu ena ngati Lombwe, atha kudzambatuka, ndikuyamba kumugenda miyala pa zomwe analembazo.
female
Masewera a AFCON, awonetsedwa pa kanema ya Super Sport. Company ya Multi-choice, yatsimikizira anthu wokonda masewero a mprira mdzikomuno.
Masewera a AFUKONI awonetsedwa pa kanema ya Supa Sipoti. kampani ya Matitchoyisi, yatsimikizira anthu wokonda masewero a mprira mdzikomuno.
female
Kuti mpira wa chakachino wa Africa Cup Of Nation (AFCON) , ukhala ukuwonetsedwa pa kanema wa Super Sport. chikalatachi chadza pamene masiku apitawa panali nkhawa,
Kuti mpira wa chakachino wa Afirika kapu Ofu Neshonzi (AFUKONI), ukhala ukuwonetsedwa pa kanema wa Supa Sipoti. chikalatachi chadza pamene masiku apitawa panali nkhawa,
female
Yoti Super Sport siwonetsa masewerowa pa kanemayu. Masewero a kalambulabwalo, ayamba loweruka likudzali, ndipo anyamata a dziko la Ivory Coast adzakhala akugwerurana mano ndi anyamata a dziko la Guinea.
Yoti Supa Sipoti siwonetsa masewerowa pa kanemayu. Masewero a kalambulabwalo, ayamba loweruka likudzali, ndipo anyamata a dziko la Ayivore Kositi adzakhala akugwerurana mano ndi anyamata a dziko la Gine.
female
Chepetsaniko zakazo, ndimadwala nthenda ya Sugar, inatero mfumu yogwiririlayo. Mfumu ina yazaka 40 ku Lilongwe, yalamulidwa kukaseweza Jere kwa zaka 20.
Chepetsaniko zakazo, ndimadwala nthenda ya Shuga, inatero mfumu yogwiririlayo. Mfumu ina yazaka fote ku Lilongwe, yalamulidwa kukaseweza Jere kwa zaka tuwente.
female
Itapezeka yolakwa pa mulandu woti idagwiririra mwana wa zaka 13 m’munda wa chimanga, pamene mwanayo ankatchola mnkhwani, atatumidwa ndi amake.
Itapezeka yolakwa pa mulandu woti idagwiririra mwana wa zaka setini m’munda wa chimanga, pamene mwanayo ankatchola mnkhwani, atatumidwa ndi amake.
female
Malingana ndi mneneri wa a police m’bomali a Hastings Chigalu ati mfumuyi yomwe dzinalake ndi a Petrous Khote, adachita zadamazi ndi mwanayu, mwezi wa June, chakachatha.
Malingana ndi mneneri wa a polisi m’bomali a Hesiting'izi Chigalu ati mfumuyi yomwe dzinalake ndi a Pitirosi Khote, adachita zadamazi ndi mwanayu, mwezi wa Juni, chakachatha.
female
Pamene mwanayu adatumidwa ndi amake, kukatchola mnkhwani m’munda. Ndipo yemwe amayimira boma pa mulanduwu a Richard Kandeya, anawuza bwalo la milanduli kuti mfumuyi idachita zadamazi ndimwanayu cha m’ma 6 m’mawa.
Pamene mwanayu adatumidwa ndi amake, kukatchola mnkhwani m’munda. Ndipo yemwe amayimira boma pa mulanduwu a Ritchadi Kandeya, anawuza bwalo la milanduli kuti mfumuyi idachita zadamazi ndimwanayu cha m’ma sikisi m’mawa.
female
Nthawi yomwe mwanayi amakathyola mnkhwani, banjalina ndilomwe lidapezerera mfumuyo ikuchita za malodzazi ndi mwanayu, koma mfumuyi idaopseza banjali.
Nthawi yomwe mwanayi amakatchola mnkhwani, banjalina ndilomwe lidapezerera mfumuyo ikuchita za malodzazi ndi mwanayu, koma mfumuyi idaopseza banjali.
female
Ponena kuti banjali lidamusokoneza zomwe amachitazo. Bwalo lamilanduli litafunsa zamulanduwo, mfumuyo idayamba ndikukana mulanduwu ponena kuti adali asanalirire mwanayo.
Ponena kuti banjali lidamusokoneza zomwe amachitazo. Bwalo lamilanduli litafunsa zamulanduwo, mfumuyo idayamba ndikukana mulanduwu ponena kuti adali asanalirire mwanayo.
female
Kenako mfumuyo inavomera mulanduwu ndikupempha bwalo la milanduli kuti limuchepetsereko zakazo, ponena kuti amadwala nthenda ya sugar. Koma bwalo lamilanduli, silidamvere dandawulo lake.
Kenako mfumuyo inavomera mulanduwu ndikupempha bwalo la milanduli kuti limuchepetsereko zakazo, ponena kuti amadwala nthenda ya shuga. Koma bwalo lamilanduli, silidamvere dandawulo lake.
female
Mpaka walamulidwa kuti akaseweze ndende kwa zaka 20, ndi cholinga choti ena atengerepo phunziro. Akathyali atatu awanjata kamba koyendetsa champeni lamya za anafedwa pamaliro.
Mpaka walamulidwa kuti akaseweze ndende kwa zaka tuwente, ndi cholinga choti ena atengerepo phunziro. Akathyali atatu awanjata kamba koyendetsa champeni lamya za anafedwa pamaliro.
female
Akathyali atatu akwidzigwidwa ndi a police ku Lilongwe kamba kowaganizira kuti anayendetsa champeni lamya za m’manja za anafedwa pamaliro, dzulo m’mudzi wa Kamganga.
Akathyali atatu akwidzigwidwa ndi a polisi ku Lilongwe kamba kowaganizira kuti anayendetsa champeni lamya za m’manja za anafedwa pamaliro, dzulo m’mudzi wa Kamganga.
female
Kwa mfumu yayikulu Mavwere m’boma la Mchinji. Nkhani yonse ikuti, akathyali atatuwa omwe mayina awo ndi a Steven Mofolo a zaka 21, a Andrew Manase azaka 28.
Kwa mfumu yayikulu Mavwere m’boma la Mchinji. Nkhani yonse ikuti, akathyali atatuwa omwe mayina awo ndi a Sitivini Mofolo a zaka tuwente-wani, a Anduru Manase azaka tuwente-eyiti.
female
Komanso a Innocent Phiri azaka 43, dzulo lachinayi akathyaliwa, adabera anafedwa lamya za m’manja pa maliro. A police owona zofufuzafufuza kuchokera kunthambi yaying’ono ya Chitipi.
Komanso a Inosenti Phiri azaka fote-firi, dzulo lachinayi akathyaliwa, adabera anafedwa lamya za m’manja pa maliro. A polisi owona zofufuzafufuza kuchokera kunthambi yaying’ono ya Chitipi.
female
Anakwanitsa kunjata akathyali atatuwa pa chipatala chachikulu cha Kamuzu Central Hospital ndi kusokolotsaso ma lamya anayi komanso kachipangizo kosungiramo mphavu zamagetsi, pachingerezi power bank.
Anakwanitsa kunjata akathyali atatuwa pa chipatala chachikulu cha Kamuzu Senturo Hosipito ndi kusokolotsaso ma lamya anayi komaso kachipangizo kosungiramo mphavu zamagetsi, pachingerezi pawa banki.
female
Malingana ndi mneneri wa a police a constable Khumbo Sanyiwa, wati akathyali atatuwa pompano akawonekera kubwalo la milandu, komwe akayankhe pa mulandu wokuba katundu.
Malingana ndi mneneri wa a polisi a consitabo Khumbo Sanyiwa, wati akathyali atatuwa pompano akawonekera kubwalo la milandu, komwe akayankhe pa mulandu wokuba katundu.
female
A Innocent Phiri ndi a m’mudzi mwa Chilumba kwa mfumu yayikulu Mnsamala ku Balaka. A Andrew Manase amachokera m’mudzi mwa gowero.
A Inosenti Phiri ndi a m’mudzi mwa Chilumba kwa mfumu yayikulu Mnsamala ku Balaka. A Anduru Manase amachokera m’mudzi mwa gowero.
female
Kwa mfumu yayikulu Chikumbu m’boma la Mulanje, pamene a Steven Mofolo, amachokera m’mudzi mwa Ngulanga kwa Likoswe ku Chiradzulu.
Kwa mfumu yayikulu Chikumbu m’boma la Mulanje, pamene a Sitivini Mofolo, amachokera m’mudzi mwa Ngulanga kwa Likoswe ku Chiradzulu.
female
Wanjatidwa kamba kogwiririra ana atatu azaka zinayi. Mnyamatawina wopanda dambisi wazaka 18, wavekedwa zibangiri ndi kusungidwa mkambolimboli ndi apolice m’boma la Thyolo.
Wanjatidwa kamba kogwiririra ana atatu azaka zinayi. Mnyamatawina wopanda dambisi wazaka eyitini, wavekedwa zibangiri ndi kusungidwa mkambolimboli ndi apolice m’boma la Thyolo.
female
Kamba komuganizira kuti adagwirira ana akazi atatu azaka zinayi zakubadwa. Nkhani yonse ikiti mnyamatayu, yemwe dzinalake ndi Milward Stanley.
Kamba komuganizira kuti adagwirira ana akazi atatu azaka zinayi zakubadwa. Nkhani yonse ikiti mnyamatayu, yemwe dzinalake ndi Miliwadi Sitanile.
female
Anachita zadamazi ndi ana atatuwa dzana pa 17 January, chakumtsinje wa Namichimba, komwe adakumana ndi anawa chakumadzulo.
Anachita zadamazi ndi ana atatuwa dzana pa seventini Januwale, chakumtsinje wa Namichimba, komwe adakumana ndi anawa chakumadzulo.
female
Mkuluyo adakokera anawa m’munda wachimanga wina ndikuyamba kuwachita zadamazi. Mnyamawina wachichepere adava kusisima m’mundamo, zomwe zinamudabwitsa mpaka adalowa m’mundamo kuti akawone.
Mkuluyo adakokera anawa m’munda wachimanga wina ndikuyamba kuwachita zadamazi. Mnyamawina wachichepere adava kusisima m’mundamo, zomwe zinamudabwitsa mpaka adalowa m’mundamo kuti akawone.
female
Apa mpamene adapeza Stanley, akuchita zakuluakulu ndi anawo. Pakadali pano yemwe ndi wachiwiri kwa mneneri wa police m’bomali a Rabecca Kashoti, watsimikiza za nkhaniyi.
Apa mpamene adapeza Sitanile, akuchita zakuluakulu ndi anawo. Pakadali pano yemwe ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi m’bomali a Rabeka Kashoti, watsimikiza za nkhaniyi.
female
Mnyamatayo, amachokera m’mudzi mwa Chibwana kwa mfumu yayikulu Mchiramwera, m’boma lomweri la Thyolo. Ndipo posachedwapa akawonekera m’bwalo la milandu pa mulandu wogwiririra
Mnyamatayo, amachokera m’mudzi mwa Chibwana kwa mfumu yayikulu Mchiramwera, m’boma lomweri la Thyolo. Ndipo posachedwapa akawonekera m’bwalo la milandu pa mulandu wogwiririra.
female
Akuluakulu woyendetsa team ya Wanderes, awachotsa. Zatsimikizika kuti mamembala a Board ya team ya mpira wamiyendo ya Mighty Mukuru Wanderes, awachotsa.
Akuluakulu woyendetsa timu ya Wandarazi, awachotsa. Zatsimikizika kuti mamembala a Bodi ya timu ya mpira wamiyendo ya Mayite Mukuru Wandarazi, awachotsa.
female
Wapampando wa timuyi a Thomson Mpinganjira, atsimikiza za nkhaniniyi. Muchikalata chomwe wasayina ndi mtsogoleriyu.
Wapampando wa timuyi a Thomusoni Mpinganjira, atsimikiza za nkhaniniyi. Muchikalata chomwe wasayina ndi mtsogoleriyu.
female
Chikufotokoza kuti izi zadza, kamba ka maganizo akuluakulu omwe ndi eni ma company omwe amathandizira kuyendetsa timuyi. Kamba kakusinthidwa kwa adindowa, chilichose choyenera kuti board ichitepo kanthu,
Chikufotokoza kuti izi zadza, kamba ka maganizo akuluakulu omwe ndi eni ma kampani omwe amathandizira kuyendetsa timuyi. Kamba kakusinthidwa kwa adindowa, chilichose choyenera kuti bodi ichitepo kanthu,
female
Chikuyenera kupita kwa Roosevelt Mpinganjira, yemwe ndi mkhalapampando mu uphunguwu. Mamembala onse omwe achotsedwa, akuyenera kukawonekera kwa mkhalapampando wa board, kuti pakhale kukozanso.
Chikuyenera kupita kwa Ruzieveti Mpinganjira, yemwe ndi mkhalapampando mu uphunguwu. Mamembala onse omwe achotsedwa, akuyenera kukawonekera kwa mkhalapampando wa bodi, kuti pakhale kukozanso.
female
Mbali imodzi yakufotokozera kwa chikalatachi. Mighty Mukuru Wanmderes ndi team yomwe yamaliza chakachonse cha 2023, osatenga chikho chilichonse, ndipo yemwe anali mphunzitsi wamkulu mu timuyi Mr Mark Harrison,
Mbali imodzi yakufotokozera kwa chikalatachi. Mayite Mukuru Wandarazi ndi timu yomwe yamaliza chakachonse cha utwente tuwente firi, osatenga chikho chilichonse, ndipo yemwe anali mphunzitsi wamkulu mu timuyi Misita Maki Harisoni,
female
Anasiya ntchito kumapeto a chakachatha, kamba kolephera kutenga chikho. Bottoman wati, akudikira chibaluwa chosonyeza kuti amuchotsa mchipani.
Anasiya ntchito kumapeto a chakachatha, kamba kolephera kutenga chikho. Botomani wati, akudikira chibaluwa chosonyeza kuti amuchotsa mchipani.
female
Mmodzi mwa anthu omwe athamangotsidwa mchipani chotsutsa boma cha DPP, Mark Bottoman, wati zoti iyie amuchotsa mchipanichi, akungowerenga mmasamba a mchenzo.
Mmodzi mwa anthu omwe athamangotsidwa mchipani chotsutsa boma cha DIPIPI, Maki Botomani, wati zoti iyie amuchotsa mchipanichi, akungowerenga mmasamba a mchenzo.
female
Ndipo iye wati akudikira kalata yochokera kuchipanichi, yosonyeza kuti amuchotsa, asanapange chiganizo chake pa nkhaniyi.
Ndipo iye wati akudikira kalata yochokera kuchipanichi, yosonyeza kuti amuchotsa, asanapange chiganizo chake pa nkhaniyi.
female
A Bottoman ati, ngakhale iwo ali ndi chikhulupiriro kuti chikalata chomwe chatuluka chochotsa anthu mchipanichi ndi chenicheni, iwo atemetsa nkhwangwa pamwala, kuti adikira kalata yawo kuchokera kuchipani yosonyeza kuti awachotsa.
A Botomani ati, ngakhale iwo ali ndi chikhulupiriro kuti chikalata chomwe chatuluka chochotsa anthu mchipanichi ndi chenicheni, iwo atemetsa nkhwangwa pamwala, kuti adikira kalata yawo kuchokera kuchipani yosonyeza kuti awachotsa.
female
A Mark Bottoman, omwenso ndi phungu wadera la Zomba, anafotokozanso kuti zoti awachotsa mchipanichi, akungowerenga m’masamba a mchenzo.
A Maki Botomani, omwenso ndi phungu wadera la Zomba, anafotokozanso kuti zoti awachotsa mchipanichi, akungowerenga m’masamba a mchenzo.
female
A Bottoman ayankhula izi, kutsatira pomwe chipanichi, chatulutsa kalata yochotsa anthu mchipani. Ndipo wa m’modzi mwa iwo ndi a Bottoman.
A Botomani ayankhula izi, kutsatira pomwe chipanichi, chatulutsa kalata yochotsa anthu mchipani. Ndipo wa m’modzi mwa iwo ndi a Botomani.
female
Zipatala zinayi zomwe zikumangidwa ku Neno, zichepetsa mavuto azawumoyo. Boma mothandizidwa ndi bungwe la Global Fund, likumanga zipatala zinayi zing’onozing’ono m’boma la Neno.
Zipatala zinayi zomwe zikumangidwa ku Neno, zichepetsa mavuto azawumoyo. Boma mothandizidwa ndi bungwe la Gulobo Fandi, likumanga zipatala zinayi zing’onozing’ono m’boma la Neno.
female
Zipatalazi, zikumangidwa kumadera ovuta kufikirako, omwe ali kutali kwambiri ndi zipatala zaboma. Zipatala zomwe zikumangidwazi ndi Gonthi, Godeni, Felemu ndi Kambale.
Zipatalazi, zikumangidwa kumadera ovuta kufikirako, omwe ali kutali kwambiri ndi zipatala zaboma. Zipatala zomwe zikumangidwazi ndi Gonthi, Godeni, Felemu ndi Kambale.
female
Ndipo zikumangidwa ndi ndalama zosachepera 1,000,000,000 kwacha. Poyankhula ndi Malawi 24, mayi m’modzi wochokera m’mudzi mwa Felemu, Afiness Felemu anati ndiwokondwa ndikubwera kwa chipatalachi.
Ndipo zikumangidwa ndi ndalama zosachepera wani biliyoni kwacha. Poyankhula ndi Malawi tuwente-folo, mayi m’modzi wochokera m’mudzi mwa Felemu, Afinesi Felemu anati ndiwokondwa ndikubwera kwa chipatalachi.
female