audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Iwo apatiriza kutsutsa mphekesera zonena kuti gulu lawo lagulitsidwa ku chipachi chomwe sanachitchure dzina. Pa chochitikachi, ena mwa amene anali nawo ndi mkulu wa Mulhako wa Alhomwe Pius Mvenya,
Iwo apatiriza kutsutsa mphekesera zonena kuti gulu lawo lagulitsidwa ku chipachi chomwe sanachitchure dzina. Pa chochitikachi, ena mwa amene anali nawo ndi mkulu wa Mulakho wa Alomwe Piysi Mvenya,
Female
Felix Namagoya yemwe ndi wapampando mu chigawo cha kumwera komaso Felix Tambulasi yemwe ndi loya. Zoti mwezi wa January umakhala ndi masiku ochuluka zedi
Felikisi Namagoya yemwe ndi wapampando mu chigawo cha kumwera komaso Felikisi Tambulasi yemwe ndi loya. Zoti mwezi wa Januwale umakhala ndi masiku ochuluka zedi
Female
oyimba ambiri siziwakhudza kamba koti bungwe la COSOMA lawaombola powapatsa dipo la thukuta lawo
oyimba ambiri siziwakhudza kamba koti bungwe la KOSOMA lawaombola powapatsa dipo la thukuta lawo
Female
komatu awiri obadwa m’ma 2000-wa asadabuza achiyamba kale poti ndiomwe atapa phwamwamwa. Lero Lachitatu, Bungwe la Copyright Society of Malawi (COSOMA)
komatu awiri obadwa m’ma Thusauzandewa-wa asadabuza achiyamba kale poti ndiomwe atapa phwamwamwa. Lero Lachitatu, Bungwe la kopelayiti sosayate ofu Malawi (KOSOMA)
Female
lagawa ndalama zokwana K505 million kwa anthu aluso mdziko muno ndipo mwa ndalamazi, K279 million ndizomwe zigawidwe kwa oyimba nyimbo
lagawa ndalama zokwana Faifi handiledi andi faifi miliyoni kwacha kwa anthu aluso mdziko muno ndipo mwa ndalamazi, thu handiledi andi seventenaini miliyoni kwacha ndizomwe zigawidwe kwa oyimba nyimbo
Female
pomwe olemba ma buku alandira K139 Million ndipo akonzi a kanema osiyanasiyana agawana K87 million
pomwe olemba ma buku alandira wani handiledi andi fete naini miliyoni kwacha ndipo akonzi a kanema osiyanasiyana agawana eyiteseveni miliyoni kwacha
Female
Pa mwambo omwe unachitikira ku hotela ya Crossroads mu mzinda wa Lilongwe, oyimba okwana 54 aliyese wapatsidwa ndalama zosachepera 1 miliyoni kwacha komaso zosapitilira 5 miliyoni Kwacha
Pa mwambo omwe unachitikira ku hotela ya Khulosilodzi mu mzinda wa Lilongwe, oyimba okwana fifitefolo aliyese wapatsidwa ndalama zosachepera wani miliyoni kwacha komaso zosapitilira faifi miliyoni Kwacha
Female
potengera chikoka cha nyimbo zawo mchaka cha 2023 chomwe changothachi. Poyankhula pa mwambowu, Driemo yemwe anabadwa Shaffie Phiri walangiza oyimba omwe sanachite bwino
potengera chikoka cha nyimbo zawo mchaka cha twente twente fili chomwe changothachi. Poyankhula pa mwambowu, Diliyemo yemwe anabadwa Shafi Phiri walangiza oyimba omwe sanachite bwino
Female
ndiposo walangiza oyimba anzake onse omwe apeza kanganyase kuti ndalama apezazi apangira chinthu chowoneka. Ena alandira zambiri kuposa ena, koma sizikutanthauza kuti amenewo ndi akutha kwambiri kuposa enawo, ayi

Zikungotanthauza kuti panopa itha kukhala nthawi ya wina wake koma kutsogoloku idzakhalaso nthawi ya wina. Zikungofunika kukankha. Penaso ukagwa ndi pomwe umakhala ndi chilimbikitso kuti ulimbikile

Kuchita bwino kwa ena chikuyenera kukhala chilimbikitso osati chiopsezo kwa ena. Kwa oyimba anzanga pena zimakhala zochititsa manyazi kuti panopa anthu adziwa kuti talandira chonchi komano pasapezeke kuti palibe chomwe tapanga chowoneka

Ndalama ingachepe bwanji yamba kanthu kakang’ono kena kake. Kaya uyamba chinthu choti chizikubweretsera K1000 pa sabata bola kusiyana nkukagulira chinthu choti ena atha kungokubera kuthera pompo” watelo Driemo
Ndalama ingachepe bwanji yamba kanthu kakang’ono kena kake. Kaya uyamba chinthu choti chizikubweretsera wanisauzande kwacha pa sabata bola kusiyana nkukagulira chinthu choti ena atha kungokubera kuthera pompo, watelo Diliyemo
Female
Khuda Myaba yemwe pano alibe timu yomwe akuonetsera ukatswiri wake, watutumutsa gulu pomwe wanena kuti alibe ganizo losewera mu ma timu a Mighty Mukuru Wanderers komanso FCB Nyasa Big Bullets
Khuda Myawa yemwe pano alibe timu yomwe akuonetsera ukatswiri wake, watutumutsa gulu pomwe wanena kuti alibe ganizo losewera mu ma timu a Maite Mukuru Wandilazi komanso Efusibi Nyasa Bigi Buletsi
Female
ponena kuti matimu onsewa sangakwanitse kumulipira pa mwezi. Myaba wauza tsamba lolemba nkhani za masewero la Wa Ganyu
ponena kuti matimu onsewa sangakwanitse kumulipira pa mwezi. Myawa wauza tsamba lolemba nkhani za masewero la Wa Ganyu
Female
kuti mphekesera zomwe zikumveka kuti iye akukambirana ndi akuluakulu a timu ya Wanderers komanso Bullets kuti iye alowere kumeneko sizoni ya masewero a mpira ikubwerayi, ndibodza la nkunkhuniza
kuti mphekesera zomwe zikumveka kuti iye akukambirana ndi akuluakulu a timu ya Wandilazi komanso Buletsi kuti iye alowere kumeneko sizoni ya masewero a mpira ikubwerayi, ndibodza la nkunkhuniza
Female
Osewerayu yemweso kumapeto a chaka chatha anali nkamwa nkamwa pakuchoka kwake ku timu ya Tishreen yomwe ndi ya mdziko la Syria, wati iye sangasewere matimu a kuno kumpanje
Osewerayu yemweso kumapeto a chaka chatha anali nkamwa nkamwa pakuchoka kwake ku timu ya Tishilini yomwe ndi ya mdziko la Siliya, wati iye sangasewere matimu a kuno kumpanje
Female
ponena kuti palibe timu yomwe amayiona kuti ingakwanitse kumamulipira ndalama zomwe iye amafuna pa mwezi uli onse. Ngati akundifuna ndiye kuti akuyenera kumandilipira ndalama za ku America
ponena kuti palibe timu yomwe amayiona kuti ingakwanitse kumamulipira ndalama zomwe iye amafuna pa mwezi uli onse. Ngati akundifuna ndiye kuti akuyenera kumandilipira ndalama za ku Amelika
Female
$1000 yomwe ili K1.7 miliyoni ndi ndalama zomwe ndikufuna monga malipiro. Ndawaona ochemelera timu ya Wanderers akunena kuti ndikulowa ku timu yawo ngati kuti angakwanitse kundilipira, Ili ndi bodza
wani sauzande dolazi yomwe ili wani pointi seveni miliyoni kwacha ndi ndalama zomwe ndikufuna monga malipiro. Ndawaona ochemelera timu ya Wandilazi akunena kuti ndikulowa ku timu yawo ngati kuti angakwanitse kundilipira, Ili ndi bodza
Female
watelo Myaba poyankhula ndi tsamba la Wa Ganyu. Nkhaniyi yakwiyitsa anthu ambiri okonda masewero a mpira wa miyendo mdziko muno ndipo ena mwa iwo mokwiya alemba m’masamba anchezo kudzudzula osewerayu
watelo Myawa poyankhula ndi tsamba la Wa Ganyu. Nkhaniyi yakwiyitsa anthu ambiri okonda masewero a mpira wa miyendo mdziko muno ndipo ena mwa iwo mokwiya alemba m’masamba anchezo kudzudzula osewerayu
Female
kuti uku sikuyankhula kwa bwino ponena kuti kwanu nkwanu mthengo mudalaka njoka. Asanapite ku timu ya Tishreen komwe wakhalako kuyambira mwezi wa August mpaka October, 2023
kuti uku sikuyankhula kwa bwino ponena kuti kwanu nkwanu mthengo mudalaka njoka. Asanapite ku timu ya Tishilini komwe wakhalako kuyambira mwezi wa Ogasiti mpaka Okotoba, twente twente fili
Female
Myaba amasewelera timu ya Polokwane City ya mdziko la South Africa, ndipo kuno ku mudzi poyamba anali osewera wa timu ya Moyale Barracks asanapite ku timu ya Silver Strikers mchaka cha 2018
Myawa amasewelera timu ya Polokwane site ya mdziko la Saufi afilika, ndipo kuno ku mudzi poyamba anali osewera wa timu ya Moyale Balakisi asanapite ku timu ya Siliva Sitilaikazi mchaka cha twente eitini
Female
Tidzalemekeza voti ya aliyense – chatero chipani cha EEFP A Griffin Maruwasa, omwe ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha ndale
Tidzalemekeza voti ya aliyense – chatero chipani cha i,iyefupi A Gilifini Maruwasa, omwe ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha ndale
Female
chomwe chikhadzikitsidwe posachedwapa cha Economic Freedom Party (EFP) atsindika kuti chipani chawo chidzawonetsetsa kuti voti ya anthu ikulemekezedwa
chomwe chikhadzikitsidwe posachedwapa cha ikonomiki fulidomu pate (iyefupi) atsindika kuti chipani chawo chidzawonetsetsa kuti voti ya anthu ikulemekezedwa
Female
A Maruwasa anena izi poyankhulana ndi Malawi24 pakutha pa mkumano omwe adali nawo ndi mamembala a chipanichi m’boma la Balaka
A Maruwasa anena izi poyankhulana ndi Malawi twente folo pakutha pa mkumano omwe adali nawo ndi mamembala a chipanichi m’boma la Balaka
Female
Iwo adati kwa nthawi yaitaili, zipani za ndale mdziko muno zakhala zikulonjeza malonjezo ambiri pa misonkhano yokopa anthu
Iwo adati kwa nthawi yaitaili, zipani za ndale mdziko muno zakhala zikulonjeza malonjezo ambiri pa misonkhano yokopa anthu
Female
ngakhale ati zipanizi zikalowa m’boma sizikwanilitsa mkomwe mfundo za mu malonjezo awo. Kuyambira mu chaka cha 1994, zipani zandale zosiyanasiyana zakhala zikubweletsa mfundo zawo zokopa anthu
ngakhale ati zipanizi zikalowa m’boma sizikwanilitsa mkomwe mfundo za mu malonjezo awo. Kuyambira mu chaka cha naintini nainte folo, zipani zandale zosiyanasiyana zakhala zikubweletsa mfundo zawo zokopa anthu
Female
Komabe, atsogoleri ake amaiwala malonjezo awo mu nthawi yokopa anthu akangolowa m’boma. Uku ndi kulakwa kwambiri
Komabe, atsogoleri ake amaiwala malonjezo awo mu nthawi yokopa anthu akangolowa m’boma. Uku ndi kulakwa kwambiri
Female
chifukwa zimasonyeza kusalabadira komanso kusalemekeza voti ya anthu adafotokoza Maruwasa. A Maruwasa adawonjezeranso kunena kuti chipani chawo sichili pa changu kulowa m’boma posachedwapa
chifukwa zimasonyeza kusalabadira komanso kusalemekeza voti ya anthu adafotokoza Maruwasa. A Maruwasa adawonjezeranso kunena kuti chipani chawo sichili pa changu kulowa m’boma posachedwapa
Female
koma anenetsa kuti Iwo ali okonzeka kugwira ntchito ndi chipani chandale chilichonse chomwe chidzawonetse chidwi komanso kuthekera kovomeleza mfundo zomwe chipani cha EFP chizakhadzikitse
koma anenetsa kuti Iwo ali okonzeka kugwira ntchito ndi chipani chandale chilichonse chomwe chidzawonetse chidwi komanso kuthekera kovomeleza mfundo zomwe chipani cha iyefupi chizakhadzikitse
Female
Malingana ndi a Maruwasa, chipani chawo chidzawonetsetsa kuti chikuika mfundo zokomera onse makamaka achinyamata, amai komanso okalamba
Malingana ndi a Maruwasa, chipani chawo chidzawonetsetsa kuti chikuika mfundo zokomera onse makamaka achinyamata, amai komanso okalamba
Female
omwe azalimbikitsidwe komanso kupatsidwa danga lotukula dziko lino kudzera mu ntchito zachitukuko zosiyanasiyana
omwe azalimbikitsidwe komanso kupatsidwa danga lotukula dziko lino kudzera mu ntchito zachitukuko zosiyanasiyana
Female
A Maruwasa adatinso Padakali pano, zonse zokonzekera kukhadzikitsa chipanichi zili mchimake. Ka chakudya tili nakoko tigawane, atero a Chakwera
A Maruwasa adatinso Padakali pano, zonse zokonzekera kukhadzikitsa chipanichi zili mchimake. Ka chakudya tili nakoko tigawane, atero a Chakwera
Female
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera apempha a Malawi kuti akondane pogawana ka chakudya kochepa kamene anthu ali nako mu nyengo ya njala ino yomwe imakhala miyezi yovuta kawirikawiri
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazalasi Chakwera apempha a Malawi kuti akondane pogawana ka chakudya kochepa kamene anthu ali nako mu nyengo ya njala ino yomwe imakhala miyezi yovuta kawirikawiri
Female
Poyankhula lero Ku Dowa pa bwalo la Andrew Murray ku Mvera Poyankhula lero Ku Dowa pa bwalo la Andrew Murray ku Mvera atayendera Nyumba zomwe zikumangidwa za asilikali a nkhondo
Poyankhula lero Ku Dowa pa bwalo la andulu mule ku Mvera Poyankhula lero Ku Dowa pa bwalo la Andulu mule ku Mvera atayendera Nyumba zomwe zikumangidwa za asilikali a nkhondo
Female
ku Mvera Support Batallion mu ulendo opita ku Salima, a Chakwera ati mkofunika kugwirana dzanja kuti tidutse m’nyengo ya mdimayi pogawana kamene kangapezekeko
ku Mvera Sapoti bataliyoni mu ulendo opita ku Salima, a Chakwera ati mkofunika kugwirana dzanja kuti tidutse m’nyengo ya mdimayi pogawana kamene kangapezekeko
Female
Lero ndi nthawi yokuti aliyense agwire dzanja la mzake mkumanena kuti tiyeni tiolokere limodzi
Lero ndi nthawi yokuti aliyense agwire dzanja la mzake mkumanena kuti tiyeni tiolokere limodzi
Female
lero ndi nthawi yakuti aliyense awonetsetse kuti tigwire ntchito molimbika kuti mawa likhale losiyana ndi m’mene dzulo linalili komanso m’mene lero lilili pakuti dzikoli tilibenso lina kwina lathu ndi lomweli

atero a Chakwera. Mtsogoleriyu wati mpofunika kuchita zofunikira kuti dzikoli likhale losinthika monga m’mene likusinthikira pakali pano
atero a Chakwera. Mtsogoleriyu wati mpofunika kuchita zofunikira kuti dzikoli likhale losinthika monga m’mene likusinthikira pakali pano
Female
M’mawu ake, Mfumu yayikulu Chiwere ya M’bomali ati ku Dowa Njala yafika povuta kwambiri ndipo apempha kuti chimanga chidzifikira mowirikiza ku delali kuti anthu apulumuke
M’mawu ake, Mfumu yayikulu Chiwere ya M’bomali ati ku Dowa Njala yafika povuta kwambiri ndipo apempha kuti chimanga chidzifikira mowirikiza ku delali kuti anthu apulumuke
Female
Mfumu Chiwere yatinso boma liganizile msanga ndondomeko yotapa Madzi ku Nyanja ya Malawi kupita ku Lilongwe ya Salima Lilongwe water project kuti ichite machawi kuti anthu a ku m’mawa kwa Dowa
Mfumu Chiwere yatinso boma liganizile msanga ndondomeko yotapa Madzi ku Nyanja ya Malawi kupita ku Lilongwe ya Salima Lilongwe wota pulojekiti kuti ichite machawi kuti anthu a ku m’mawa kwa Dowa
Female
apindulenso pakuti mdelali madzi ndi ovuta kuwapeza. Phungu wa delali a Richard Chimwendo Banda mmau ake anati dela lake ndi lokwera kotero mijigo sitheka
apindulenso pakuti mdelali madzi ndi ovuta kuwapeza. Phungu wa delali a Ritchadi Chimwendo Banda mmau ake anati dela lake ndi lokwera kotero mijigo sitheka
Female
ndipo anagwirizana ndi a Chiwere kuti ndondomeko yotapa Madzi ku Salima ikhala yofunika kwambiri kwa anthu a delali
ndipo anagwirizana ndi a Chiwere kuti ndondomeko yotapa Madzi ku Salima ikhala yofunika kwambiri kwa anthu a delali
Female
Anthu 7 apezeka ndi kachirombo ka Covid-19 ku Nsanje. Pomwe anthu ochuluka anayamba kuiwala za matenda a Covid-19, zadziwika kuti matendawa anakalipo mdziko muno
Anthu seveni apezeka ndi kachirombo ka Kovidi-naintini ku Nsanje. Pomwe anthu ochuluka anayamba kuiwala za matenda a Kovidi-naintini, zadziwika kuti matendawa anakalipo mdziko muno
Female
pomwe ku Nsanje akuti anthu asanu ndi awiri 7, apezeka ndi kachirombo koyambitsa matendawa. Izi ndi malingana ndi a George Mbotwa
pomwe ku Nsanje akuti anthu asanu ndi awiri seveni, apezeka ndi kachirombo koyambitsa matendawa. Izi ndi malingana ndi a Joji Mbotwa
Female
omwe ndi m’modzi mwa akuluakulu ku ofesi ya zaumoyo m’boma la Nsanje omwe atsimikizira nyumba zina zofalitsa nkhani mdziko muno zokhudza nkhaniyi
omwe ndi m’modzi mwa akuluakulu ku ofesi ya zaumoyo m’boma la Nsanje omwe atsimikizira nyumba zina zofalitsa nkhani mdziko muno zokhudza nkhaniyi
Female
Malingana ndi a Mbotwa, anthu asanu ndi awiriwa apezeka ndi kachirombo koyambitsa matenda a Covid-19 apezeka ndi kachirombo koyambitsa matenda a Covid-19
Malingana ndi a Mbotwa, anthu asanu ndi awiriwa apezeka ndi kachirombo koyambitsa matenda a Kovidi-naintini apezeka ndi kachirombo koyambitsa matenda a Kovidi-naintini
Female
kumathero a sabata yomwe yangothayi pomwe anayezedwa potsatira kuonetsa zizindikiro za matendawa. Tsamba lino lapeza kuti anthu asanu ndi m’modzi 6
kumathero a sabata yomwe yangothayi pomwe anayezedwa potsatira kuonetsa zizindikiro za matendawa. Tsamba lino lapeza kuti anthu asanu ndi m’modzi sikisi
Female
mwa omwe akudwala matendawa, apezeka pa chipatala chaching’ono cha Kalemba, pomwe pa chipatala chachikulu cha Nsanje, papezeka munthu odwala matenda a Covid-19 m’modzi
mwa omwe akudwala matendawa, apezeka pa chipatala chaching’ono cha Kalemba, pomwe pa chipatala chachikulu cha Nsanje, papezeka munthu odwala matenda a Kovidi-naintini m’modzi
Female
Pakadali pano, zikumveka kuti ofesi ya zaumoyo m’bomali, yayitanitsa mkumano wa dzidzidzi kuti akuluakulu a zaumoyo m’bomali
Pakadali pano, zikumveka kuti ofesi ya zaumoyo m’bomali, yayitanitsa mkumano wa dzidzidzi kuti akuluakulu a zaumoyo m’bomali
Female
akakambirane za njira zomwe angatsate pofuna kuthana ndi kufalikira kwa matendawa m’boma lawo. Matenda a Covid-19 omwe anayambira mdziko la China mchaka cha 2019
akakambirane za njira zomwe angatsate pofuna kuthana ndi kufalikira kwa matendawa m’boma lawo. Matenda a Kovidi-naintini omwe anayambira mdziko la China mchaka cha twente naintini
Female
amayambitsidwa ndi kachilombo kotchedwa kolona (coronavirus) ndipo matendawa apha anthu ochuluka mdziko muno komaso maiko ochuluka pa dziko la pansi
amayambitsidwa ndi kachilombo kotchedwa kolona (kolona vailasi) ndipo matendawa apha anthu ochuluka mdziko muno komaso maiko ochuluka pa dziko la pansi
Female
Zina mwa njira zopewera matendawa ndi monga kusamba m’manja ndi sopo pafupifupi, kuvala zozitchinjilizira kukamwa komaso kupewa kuyandikana kapena kukhudzana mwachisawawa ndi anthu odwala matendawa

Boma latsindika kuti limanga mabwalo amasewera a Bullets ndi Wanderers. Boma latsindika ku mtundu wa a Malawi
Boma latsindika kuti limanga mabwalo amasewera a Buletsi ndi Wandilazi. Boma latsindika ku mtundu wa a Malawi
Female
kuti limanga mabwalo amasewero a matimu a Mighty Mukuru Wanderers komanso FCB Nyasa Big Bullets mu mzinda wa Blantyre
kuti limanga mabwalo amasewero a matimu a Maite Mukuru Wandilazi komanso Efusibi Nyasa Bigi Buletsi mu mzinda wa Bulantaya
Female
Nduna yoona za achinyamata ndi masewero mdziko muno a Uchizi Mkandawire ndi omwe atsindika za nkhaniyi. Ntchito yomanga mabwalo amasewerawa
Nduna yoona za achinyamata ndi masewero mdziko muno a Uchizi Mkandawire ndi omwe atsindika za nkhaniyi. Ntchito yomanga mabwalo amasewerawa
Female
alnaengezedwa koyamba mchaka cha 2020 koma idayamba yayima kaye. Kotero ndunayi yatsindika ku mtundu wa a Malawi kuti ntchitoyi iyambiranso mpaka kufika poti yatha moyenera
alnaengezedwa koyamba mchaka cha twente twente koma idayamba yayima kaye. Kotero ndunayi yatsindika ku mtundu wa a Malawi kuti ntchitoyi iyambiranso mpaka kufika poti yatha moyenera
Female
Boma lanena izi kutsatira lonjezo lomwe mboyomu lidalonjeza kuti limanga mabwalo amasewerowa. Zokambirana zikuyembekezeka kukavuta ku nyumba ya malamulo
Boma lanena izi kutsatira lonjezo lomwe mboyomu lidalonjeza kuti limanga mabwalo amasewerowa. Zokambirana zikuyembekezeka kukavuta ku nyumba ya malamulo
Female
Pamene nyumba ya malamulo ya dziko lino yatsala ndi masiku wochepa kuti iyambe zokambirana zake, pali kuthekera kuti zokambirana mnyumbayi zitha kukhala zovuta
Pamene nyumba ya malamulo ya dziko lino yatsala ndi masiku wochepa kuti iyambe zokambirana zake, pali kuthekera kuti zokambirana mnyumbayi zitha kukhala zovuta
Female
Izi zili chomwechi kutsatira chiganizo chomwe Sipikala wa nyumbayi a Catherine Gotani Hara molangizidwa ndi mkulu wa zamalamulo ku boma a Thabo Nyirenda
Izi zili chomwechi kutsatira chiganizo chomwe Sipikala wa nyumbayi a Kafelini Gotani Hara molangizidwa ndi mkulu wa zamalamulo ku boma a Thabo Nyirenda
Female
apanga posavomereza kusankhidwa kwa a George Chaponda ngati mtsogoleri wa otsutsa kunyumba ya malamulo
apanga posavomereza kusankhidwa kwa a Joji Chaponda ngati mtsogoleri wa otsutsa kunyumba ya malamulo
Female
Chipani chachikulu chotsutsa cha cha Democratic Progressive (DPP) anthu ena mchipanicho ndipo mmodzi mwa iwo ndi a Kondwani Nankhumwa
Chipani chachikulu chotsutsa cha cha Demokatatiki pulogilesivi (Dipipi) anthu ena mchipanicho ndipo mmodzi mwa iwo ndi a Kondwani Nankhumwa
Female
Chipanichi chinasankha a Dr George Chaponda pa undindo wa mtsogoleri wotsutsa boma. Kudzera mukalata yake, DPP inadziwitsa sipikaa wa nyumba ya malamulo Catherine Gotani Hara
Chipanichi chinasankha a Dokota Joji Chaponda pa undindo wa mtsogoleri wotsutsa boma. Kudzera mukalata yake, Dipipi inadziwitsa sipikaa wa nyumba ya malamulo Cafelini Gotani Hara
Female
Ndipo Pa 29, January,2024, Sipikala wa nyumba yamalamuloyi anaziwitsa chipani cha DPP kuvomeleza za kusankhidwa kwa a Chaponda ngati mtsogoleri wa wotsutsa
Ndipo Pa twente naini, Januwale, twente twernte folo, Sipikala wa nyumba yamalamuloyi anaziwitsa chipani cha Dipipi kuvomeleza za kusankhidwa kwa a Chaponda ngati mtsogoleri wa wotsutsa
Female
ndipo iwo anafunilaso mafuno abwino a Chaponda posankhidwa pa udindowu. Ndipo kalatayo inapitiliza kupempha a Chaponda
ndipo iwo anafunilaso mafuno abwino a Chaponda posankhidwa pa udindowu. Ndipo kalatayo inapitiliza kupempha a Chaponda
Female
kuti akupemphedwa kudzakhala nawo pa zokambirana za komiti yayikulu yowona zokambirana za aphungu mnyumbayo womwe uzakhalepo lachiwiri pa 6 February 2024 nthawi ya 9:30 Mamawa
kuti akupemphedwa kudzakhala nawo pa zokambirana za komiti yayikulu yowona zokambirana za aphungu mnyumbayo womwe uzakhalepo lachiwiri pa sikisi febuluwale twente twente folo nthawi ya hafu pasiti naini Mamawa
Female
Koma maloya a Nankhumwa analembela ofesi ya sipikala kuti a Nakhumwa akadalibe pa udindo wawo ngati Mtsogoleri wotsutsa boma ndiye kuvomeleza a Chaponda kukhala kuphwanya malamulo
Koma maloya a Nankhumwa analembela ofesi ya sipikala kuti a Nakhumwa akadalibe pa udindo wawo ngati Mtsogoleri wotsutsa boma ndiye kuvomeleza a Chaponda kukhala kuphwanya malamulo
Female
Mukudziwa kuti pali chiletso chomwe a Nankhumwa anakatenga ku bwalo la milandu m’mbuyomu chomwe sichinachotsedwe, kotero kuvomereza a Chaponda kukhala kudelera khoti lomwe linapereka chiletsocho, panthawi ya m’mbuyomu,

anatelo woyimilira a Nankhumwa. Ndipo Mlangizi wa boma pa zamalamulo a Thabo Chakaka Nyirenda alangiza sipikala wa nyumba ya malamulo, kuti ofesi yake isavomeleze
anatelo woyimilira a Nankhumwa. Ndipo Mlangizi wa boma pa zamalamulo a Thabo Chakaka Nyirenda alangiza sipikala wa nyumba ya malamulo, kuti ofesi yake isavomeleze
Female
a Chaponda ngati mtsogoleri watsopano wa mbali yotsutsa. Koma akatswiri pa nkhani za ndale ndi malamulo akuti a Nankhumwa sali woyenera kukhala mtsogoleri wotsutsa boma mnyumbayo
a Chaponda ngati mtsogoleri watsopano wa mbali yotsutsa. Koma akatswiri pa nkhani za ndale ndi malamulo akuti a Nankhumwa sali woyenera kukhala mtsogoleri wotsutsa boma mnyumbayo
Female
ponena kuti chipani ndichomwe chili ndi mphamvu yosankha mtsogoleri wotsutsa. Akatswiriwo alangiza a Nankhumwa kuti avomeleze kuti iwo simembelaso wachipani cha DPP
ponena kuti chipani ndichomwe chili ndi mphamvu yosankha mtsogoleri wotsutsa. Akatswiriwo alangiza a Nankhumwa kuti avomeleze kuti iwo simembelaso wachipani cha Dipipi
Female
Koma katswili wina pa za malamulo George Jivason Kazipatike wati ngati kubwalo la za milandu kuli chiletso ndiye kuti a Nankhumwa akadali mtsogoleri wotsutsa
Koma katswili wina pa za malamulo Joji Jivasoni Kazipatike wati ngati kubwalo la za milandu kuli chiletso ndiye kuti a Nankhumwa akadali mtsogoleri wotsutsa
Female
A Kazipatike ati chipani cha DPP chiyenera kukachotsa chiletsocho. Ndisimike pano kuti ndizoona kuti chipani chili ndi mphamvu zosankha mtsogoleri wotsutsa mnyumba ya malamulo
A Kazipatike ati chipani cha DPP chiyenera kukachotsa chiletsocho. Ndisimike pano kuti ndizoona kuti chipani chili ndi mphamvu zosankha mtsogoleri wotsutsa mnyumba ya malamulo
Female
ndipo chipanicho posankha a Chaponda sichinalakwe anatero a Kazipatike poyankhula ndi Malawi24
ndipo chipanicho posankha a Chaponda sichinalakwe anatero a Kazipatike poyankhula ndi Malawi twente folo
Apolice ku Kasungu, akusunga mchitokosi njonda ina ya zaka 35, za kubadwa, kamba kopezeka ndi katundu monga wireless zakanema zinayi za mtundu wa Plasma.
Apolisi ku Kasungu, akusunga mchitokosi njonda ina ya zaka sete, za kubadwa, kamba kopezeka ndi katundu monga wayilesi zakanema zinayi za mtundu wa Pulazima.
female
Ndipo njondayi, ikuganiziridwa kuti inachita mwakuba katunduyu. Wachiwiri kwa m’neneri wa police m’bomali a Miracle Nkozi, ati njondayi yomwe dzinalake ndi a Goodson Alli.
Ndipo njondayi, ikuganiziridwa kuti inachita mwakuba katunduyu. Wachiwiri kwa m’neneri wa polisi m’bomali a Mirako Nkozi, ati njondayi yomwe dzinalake ndi a Gudusoni Ali.
female
Inapezeka ndi katunduyu kunyumba yake ku Chitete, kutsatira anthu ena atatsina khutu a police za nkhaniyi, apa a police sanazengereze, koma kuthamangira ku nyumba kwa njondayi.
Idapezeka ndi katunduyu kunyumba yake ku Chitete, kutsatira anthu ena atatsina khutu a polisi za nkhaniyi, apa a polisi sanazengereze, koma kuthamangira ku nyumba kwa njondayi.
female
Komwe anakapeza katunduyu, ndi kunjata nkuluyo. Posachedwapa njondayi ikawonekera ku bwalo la milandu ndi kukayankha mulandu wa kuba.
Komwe anakapeza katunduyu, ndi kunjata nkuluyo. Posachedwapa njondayi ikawonekera ku bwalo la milandu ndi kukayankha mulandu wa kuba.
female
Njondayi imachokera m’mudzi mwa Dzimbiri kwa mfumu yayikulu Jelasi,m’boma la Mangochi. Katswiri pa nkhani za ndale wati boma lachita chamuna pothetsa milandu ya anthu osokoneza m’dipiti.
Njondayi imachokera m’mudzi mwa Dzimbiri kwa mfumu yayikulu Jelasi,m’boma la Mangochi. Katswiri pa nkhani za ndale wati boma lachita chamuna pothetsa milandu ya anthu osokoneza m’dipiti.
female
M’modzi mwa a katswiri omwe amayankhulapo pankhani za m’dziko muno, a Laifford Chadza, ayamikira boma kamba kothetsa mulandu wa anthu atatu.
M’modzi mwa a katswiri omwe amayankhulapo pankhani za m’dziko muno, a Layifodi Chadza, ayamikira boma kamba kothetsa mulandu wa anthu atatu.
female
Omwe adanjatidwa kamba kosokoneza galimoto za m’dipiti, ponena kuti izi zidakawononga ubale wabwino pakati pa boma ndi anthu aku Ndirande.
Omwe adanjatidwa kamba kosokoneza galimoto za m’dipiti, ponena kuti izi zidakawononga ubale wabwino pakati pa boma ndi anthu aku Ndirande.
female
Malingana ndi a Chanza, ati zomwe lachita boma, ndi chiyambi chokoza ndi kumanga ubale wabwino pakati pa anthu aku Ndirande komanso boma, kamba koti izi zikadatha kusokoneza ubalewu.
Malingana ndi a Chanza, ati zomwe lachita boma, ndi chiyambi chokoza ndi kumanga ubale wabwino pakati pa anthu aku Ndirande komanso boma, kamba koti izi zikadatha kusokoneza ubalewu.
female
Katswiriyu anapitirizaso kufotokoza kuti nkofunika kupezaso njira zina zomwe zingathandizire kuyanjanitsa mbali zonse ziwiri, ndi cholinga choti pakhale ubale wabwino
Katswiriyu anapitirizaso kufotokoza kuti nkofunika kupezaso njira zina zomwe zingathandizire kuyanjanitsa mbali zonse ziwiri, ndi cholinga choti pakhale ubale wabwino
female
A Chanza ayankhula izi kutsatira nkulu woyimira boma pa mulanduwu, atalengeza kuti boma lathetsa mulandu wa anthu atatu omwe anawanjata kamba kosokoneza galimoto za pa m’dipiti wa m’tsogoleri.
A Chanza ayankhula izi kutsatira nkulu woyimira boma pa mulanduwu, atalengeza kuti boma lathetsa mulandu wa anthu atatu omwe anawanjata kamba kosokoneza galimoto za pa m’dipiti wa m’tsogoleri.
female
Pamene a Lazarus Chakwera, ankapita kukakwera ndenge pa bwalo la Chileka mu m’zinda wa Blantyre. Boma lati ligwira ntchito limodzi ndi mnyamata wakonza magetsi ku Dowa.
Pamene a Lazarasi Chakwera, ankapita kukakwera ndenge pa bwalo la Chileka mu m’zinda wa Bulantaya. Boma lati ligwira ntchito limodzi ndi mnyamata wakonza magetsi ku Dowa.
female
Boma kudzera mwa nduna yowona za magetsi mdzikomuno a Ibrahim Matola,lalonjeza kuti lithandiza mnyamata uja wakoza magetsi oyendera madzi ndi mpweya ku Dowa.
Boma kudzera mwa nduna yowona za magetsi mdzikomuno a Iburahimu Matola,lalonjeza kuti lithandiza mnyamata uja wakoza magetsi oyendera madzi ndi mpweya ku Dowa.
female
Kufikira masomphenya ake woyika magetsi pa school ya Kongwe 2, komaso nyumba za m’mudzi mwake, atakwaniritsidwa.
Kufikira masomphenya ake woyika magetsi pa sukulu ya Kongwe thu, komaso nyumba za m’mudzi mwake, atakwaniritsidwa.
female
Nduna yowona za magetsi mdzikomuno a Ibrahim Matola, ndiomwe ayankhula izi lero lachisanu, pomwe ndunayi imamuyendera Enerst Andrew, yemwe wakoza magetsiwa.
Nduna yowona za magetsi mdzikomuno a Iburahimu Matola, ndiomwe ayankhula izi lero lachisanu, pomwe ndunayi imamuyendera Enesiti Anduru, yemwe wakoza magetsiwa.
female
Kwawo ku Dowa m’mudzi wa Chinguwo kwa mfumu yayikulu Chiwere. A Matola anati, sangamukakamize mnyamatayu kuti abwerereso nkalasi,kamba koti mnyamatayu school adasiya ndi kale.
Kwawo ku Dowa m’mudzi wa Chinguwo kwa mfumu yayikulu Chiwere. A Matola anati, sangamukakamize mnyamatayu kuti abwerereso nkalasi,kamba koti mnyamatayu sukulu adasiya ndi kale.
female
Kotero a Matola anati, boma limuthandiza kuti mnyamatayu, akwaniritse masomphenya ake oyika pa school ya primary komaso m’mudzi mwawo.
Kotero a Matola anati, boma limuthandiza kuti mnyamatayu, akwaniritse masomphenya ake oyika pa sukulu ya pulayimare komaso m’mudzi mwawo.
female
Koma mnyamatayu, wapempha ndunayi kuti imuthandize kumugulira nthambo zamagetsi ndi cholinga choti akwaniritse kupala magetsiwa.
Koma mnyamatayu, wapempha ndunayi kuti imuthandize kumugulira nthambo zamagetsi ndi cholinga choti akwaniritse kupala magetsiwa.
female
Ndunayi yayendera mnyamatayu, kutsatira masiku apitawo, mnyamatayu, wakhala akuyikidwa m’masamba amchezo, kuwonetsa luso lake lapamwambali.
Ndunayi yayendera mnyamatayu, kutsatira masiku apitawo, mnyamatayu, wakhala akuyikidwa m’masamba amchezo, kuwonetsa luso lake lapamwambali.
female
DODMA, yapereka thandizo kwa anthu okhudzika ndi kusefukira kwa madzi ku Dowa. Kutsatira kusefukira kwa madzi komwe kwakhudza anthu a m’boma la Dowa ku mponera, bungwe lowona za ngozi zogwa mwadzidzidzi la DODMA.
DODIMA, yapereka thandizo kwa anthu okhudzika ndi kusefukira kwa madzi ku Dowa. Kutsatira kusefukira kwa madzi komwe kwakhudza anthu a m’boma la Dowa ku mponera, bungwe lowona za ngozi zogwa mwadzidzidzi la DODIMA.
female
Dzulo lapereka thandizo losiyanasiyana kuphatikizapo ufa, ma bulangete, ma bigiri, ma Tenti komaso nyemba.
Dzulo lapereka thandizo losiyanasiyana kuphatikizapo ufa, ma bulangete, ma bigiri, ma Tenti komaso nyemba.
female
Bungweri, lapereka ma blanget wokwana 139, ufa matumba wokwana 37, nyemba zolemera ma killogram 10 ku banja lililonse,ma Tent komaso ma bigiri wokwana 37.
Bungweri, lapereka ma bulangete wokwana wani sete-nayini, ufa matumba wokwana sete-seveni, nyemba zolemera ma killogram teni ku banja lililonse, ma Tenti komaso ma bigiri wokwana sete-seveni.
female
A Mercy Mpakule, omwe ndi wankulu woyang’anira za chitukuko ku Khonsolo ya Dowa, ayamikira bungweri, kamba kochita machawi, popereka thandizoli ndipo ati labwera nthawi yake.
A Mese Mpakule, omwe ndi wankulu woyang’anira za chitukuko ku Khonsolo ya Dowa, ayamikira bungweri, kamba kochita machawi, popereka thandizoli ndipo ati labwera nthawi yake.
female
Pamene maanja ambiri ali kunkhongo kusowa mtengo wogwira. A Mpakule anapitirizanso kuti apa npoyambira chabe, kotero omwe ali ndi kuthekera kopereka thandizo.
Pamene maanja ambiri ali kunkhongo kusowa mtengo wogwira. A Mpakule anapitirizanso kuti apa npoyambira chabe, kotero omwe ali ndi kuthekera kopereka thandizo.
female
Asazengereze, koma apite kukapereka thandizoli kudzera ku office yawo ya DODMA m’bomali. Malingana ndi a Mpakule,tsopano anthu omwe atisiya kamba ka ngoziyi ndi atatu.
Asazengereze, koma apite kukapereka thandizoli kudzera ku ofesi yawo ya DODIMA m’bomali. Malingana ndi a Mpakule,tsopano anthu omwe atisiya kamba ka ngoziyi ndi atatu.
female
Pamene maanja 37 ndi omwe akhudzidwa ndi ngoziyi, pamene nyumba ndi mbewu zakokoloka. Pakadali pano ena mwa omwe aperekako thandizo ndi a Napoleon Dzombe, omwe apereka thandizo la ufa wa phala.
Pamene maanja sete ndi omwe akhudzidwa ndi ngoziyi, pamene nyumba ndi mbewu zakokoloka. Pakadali pano ena mwa omwe aperekako thandizo ndi a Napoliyoni Dzombe, omwe apereka thandizo la ufa wa phala.
female
Mneneri Shepherd Bushiri yemwe ndi mtsogoleri wa mpingo wa ECG, Jesus Nation Church, walengeza kuti akufuna kugula ndenge yonyamula anthu obwera ku ma pemphero ake kuchokera ku maiko ena.
Mneneri Shepadi Bushiri yemwe ndi mtsogoleri wa mpingo wa ISIJI, Jizasi Neshoni Tchechi, walengeza kuti akufuna kugula ndenge yonyamula anthu obwera ku ma pemphero ake kuchokera ku maiko ena.
female
Izi ndi malingana ndi zomwe mneneriyu walemba pa tsamba lake la Facebook lero lachitatu, pomwe wati lingalilori,labwera kamba koti akuwona kuti ma company a ndenge, akumudyera masuku pa mutu.
Izi ndi malingana ndi zomwe mneneriyu walemba pa tsamba lake la Fesibuku lero lachitatu, pomwe wati lingalilori, labwera kamba koti akuwona kuti ma kampani a ndenge, akumudyera masuku pa mutu.
female