audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
Mlembi wamkulu mu unduna wazamalo, Devie Chilonga, wati undunawu ukuyembekezeka kuyamba ntchito yowunikaso malire a dziko la Malawi ndi Zambia, mwenzi wa May ndi June chakachino. | Mlembi wamkulu mu unduna wazamalo, Devi Chilonga, wati undunawu ukuyembekezeka kuyamba ntchito yowunikaso malire a dziko la Malawi ndi Zambia, mwenzi wa Meyi ndi Juni chakachino. | female | |
Chilonga wati kutsatira mfundo zomwe zinatuluka pa mgwirizano wa mbali ziwirizi, akatswiri ochita kawuniwuni wamalo, akuyembekezeka kuyamba kuwunika malire a pakati pa mayiko awiriwa. | Chilonga wati kutsatira mfundo zomwe zinatuluka pa mgwirizano wa mbali ziwirizi, akatswiri ochita kawuniwuni wamalo, akuyembekezeka kuyamba kuwunika malire a pakati pa mayiko awiriwa. | female | |
Komabe ntchitoyi, ikudikira ndalama zomwe zikuyembekezeka kuperekedwa mu ndondomeko ya chuma cha boma ya mchaka cha 2024-2025. Pankhani yokhudza malire adzikolino ndi dziko la Mozambique, | Komabe ntchitoyi, ikudikira ndalama zomwe zikuyembekezeka kuperekedwa mu ndondomeko ya chuma cha boma ya mchaka cha tuwente tuwente-folo-tuwente tuwente-fayifi. Pankhani yokhudza malire adzikolino ndi dziko la Mozambiki, | female | |
Chilonga wati undunawu ukudikira chilolezo cha unduna wowona za ubale wadzikolino ndi mayiko ena. Ndipo akuyembekeza kukhala ndi misonkhano masabata akudzawa, kuti akambirane za izi. | Chilonga wati undunawu ukudikira chilolezo cha unduna wowona za ubale wadzikolino ndi mayiko ena. Ndipo akuyembekeza kukhala ndi misonkhano masabata akudzawa, kuti akambirane za izi. | female | |
Ntchito yosindikizaso malire apakati pa mayiko a Malawi ndi Zambia, inayamba pafupifupi zaka 20, zapitazo. Mkhalapampando wa Committee yoona za umoyo wakunyumba ya malamulo, Dr. Mathews Ngwale. | Ntchito yosindikizanso malire apakati pa mayiko a Malawi ndi Zambia, inayamba pafupifupi zaka tuwente, zapitazo. Mkhalapampando wa komiti yoona za umoyo wakunyumba ya malamulo, Dokota Mafiyuzi Ngwale. | female | |
Wati ndiwokhutira ndi kukwera kwa chiwerengero cha anthu omwe akupereka maganizo awo, palingaliro lofuna kusintha lamulo, lomwe limapereka mphavu yomanga munthu yemwe amafuna kudzipha mdzikomuno. | Wati ndiwokhutira ndi kukwera kwa chiwerengero cha anthu omwe akupereka maganizo awo, palingaliro lofuna kusintha lamulo, lomwe limapereka mphavu yomanga munthu yemwe amafuna kudzipha mdzikomuno. | female | |
Dr. Ngwale, wati lamulo lomwe lilipo pakadali pano, lawonetsa kulephera pothana ndi vuto lomwe limakhudza kaganizidwe kangwiro, ndipo mpofunika kukhazikitsidwa kwa lamulo latsopano. | Dokota Ngwale, wati lamulo lomwe lilipo pakadali pano, lawonetsa kulephera pothana ndi vuto lomwe limakhudza kaganizidwe kangwiro, ndipo mpofunika kukhazikitsidwa kwa lamulo latsopano. | female | |
Lomwe lingathandizire kubweretsa kaganizidwe kangwiro pakati pa nzika zadzikolino. Iwo ati, pakadali pano, anthu ochuluka awonetsa chidwi chawo, paganizo latsopano losintha lamuloli. | Lomwe lingathandizire kubweretsa kaganizidwe kangwiro pakati pa nzika zadzikolino. Iwo ati, pakadali pano, anthu ochuluka awonetsa chidwi chawo, paganizo latsopano losintha lamuloli. | female | |
Ndipo committee, yipitiriza kukambirana komaso kumva maganizo amagulu osiyanasiyana pankhaniyi, ndikugwiritsa ntchito bwino lomwe, maganizowa akadzaunikidwa. | Ndipo komiti, yipitiriza kukambirana komaso kumva maganizo amagulu osiyanasiyana pankhaniyi, ndikugwiritsa ntchito bwino lomwe, maganizowa akadzaunikidwa. | female | |
Bungwe lophunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana la Nice Trust, likulimbikitsa zipani zandale mdzikomuno, kuti zikhazikitse ndondomeko zapadera. | Bungwe lophunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana la Nayisi Thirasiti, likulimbikitsa zipani zandale mdzikomuno, kuti zikhazikitse ndondomeko zapadera. | female | |
Zomwe zithandizire amayi omwe akufuna kudzapikisananawo pachisankho cha chaka chamawa. Mkulu wa bungweri m’boma la Kasungu Pilirani Chaguza. | Zomwe zithandizire amayi omwe akufuna kudzapikisananawo pachisankho cha chaka chamawa. Mkulu wa bungweri m’boma la Kasungu Pilirani Chaguza. | female | |
Wati mchitidwe wopereka ndalama kapena katundu kwa anthu woponya vote, umakhudza amayi nthawi ya zisankho ndipo wati ndi wochilimika pofuna kuthana ndi mchitidwewu pa zisankho zikudzazi. | Wati mchitidwe wopereka ndalama kapena katundu kwa anthu woponya vote, umakhudza amayi nthawi ya zisankho ndipo wati ndi wochilimika pofuna kuthana ndi mchitidwewu pa zisankho zikudzazi. | female | |
Mkhalapampando wa khonsolo ya boma la Kasungu yemweso ndi mayi wodziwika bwino pandale m’bomalo Mwambirazo Mbedza, wapempha bungwe loyendetsa zisankho za MEC. | Mkhalapampando wa khonsolo ya boma la Kasungu yemweso ndi mayi wodziwika bwino pandale m’bomalo Mwambirazo Mbedza, wapempha bungwe loyendetsa zisankho za MEKI. | female | |
Kuti lichilimike powonetsetsa kuti malamulo okhudza kupereka ndalama kwa anthua ovota, akugwira ntchito. Mchaka cha 2018, dziko la Malawi, lidakhazikitsa lamulo loletsa anthu andale kupereka ndalama | Kuti lichilimike powonetsetsa kuti malamulo okhudza kupereka ndalama kwa anthua ovota, akugwira ntchito. Mchaka cha tuwente eyitini, dziko la Malawi, lidakhazikitsa lamulo loletsa anthu andale kupereka ndalama | female | |
Komaso katundu wina kwa oponya voti munthawi yamisonkhano yokopa anthu, koma izi sizitsatiridwa. | Komaso katundu wina kwa oponya voti munthawi yamisonkhano yokopa anthu, koma izi sizitsatiridwa. | female | |
Team ya mpira wamiyendo ya Silver Strikers, yalengeza za kuchotsedwa ntchito kwa mphunzitsi wamkulu wa timuyi. Peter Tizyani. | Timu ya mpira wamiyendo ya Silia Sitirayikazi, yalengeza za kuchotsedwa ntchito kwa mphunzitsi wamkulu wa timuyi. Pita Tizyani. | female | |
Malingana ndi chikalata chomwe timuyi yatulutsa. Ganizoli ladza powunikira momwe timuyi yachitira pokwaniritsa ngodya zomwe anapatsidwa kuti akwaniritse. | Malingana ndi chikalata chomwe timuyi yatulutsa. Ganizoli ladza powunikira momwe timuyi yachitira pokwaniritsa ngodya zomwe anapatsidwa kuti akwaniritse. | female | |
Tizyani adayamba kugwira ntchito ngati mphunzitsi wamkulu wa timuyi, mwenzi wa February, chaka cha 2023. Timuyi yati iyamba ntchito yosaka mphunzitsi wina posachedwapa. | Tizyani adayamba kugwira ntchito ngati mphunzitsi wamkulu wa timuyi, mwenzi wa Feburuware, chaka cha tuwente tuwente-firi. Timuyi yati iyamba ntchito yosaka mphunzitsi wina posachedwapa. | female | |
Mu ulamuliro wa Tizyani, ma Bankers sadapambane chikho chilichonse, kupatula kutsirizira pa nambala ya chiwiri mu mpikisano wa TNM Super League. | Mu ulamuliro wa Tizyani, ma Bankazi sadapambane chikho chilichonse, kupatula kutsirizira pa nambala ya chiwiri mu mpikisano wa TI ENI EMU Supa Ligi. | female | |
Komanso kufika ndime yotsiriza mu mpikisano wa Castel Cup. Apolice mdziko la Nigeria, amanga mwana wa mwamuna komanso wamkazi wongomulera chabe, wa wochita zisudzo mdzikolo John Okafor. | Komanso kufika ndime yotsiriza mu mpikisano wa Ckasitelo kapu. Apolisi mdziko la Nigeria, amanga mwana wa mwamuna komanso wamkazi wongomulera chabe, wa wochita zisudzo mdzikolo Joni Okafo. | ||
Yemwe amadziwika bwino kuti Mr Ibu, powaganizira kuti aba ndalama zothandizira bambo awo kulandira thandizo la chipatala. Anawa omwe ndi Onyebushi Okafor ndi Jasimine Omike Agwu. | Yemwe amadziwika bwino kuti Misita Ibu, powaganizira kuti aba ndalama zothandizira bambo awo kulandira thandizo la chipatala. Anawa omwe ndi Onyebushi Okafo ndi Jasimine Omike Agwu. | female | |
Akuganiziridwa kuti anatenga lamya yabawo awo ndikudzitumizira ndalama zokwana 55,000,000, za mdziko la Nigeria. | Akuganiziridwa kuti anatenga lamya yabawo awo ndikudzitumizira ndalama zokwana fifite fayifi miliyoni, za mdziko la Nigeria. | female | |
Ndalamazi, zinali gawo landalama zomwe anthu akufuna kwabwino anapereka kwa Mr, Ibu, Kuti ziwathandizire ku chipatala, atadwala kwa nthawi yayitali chakachatha. Kudwalaku kudachititsa kuti Mr. Ibu, adulidwe mwendo umodzi. | Ndalamazi, zinali gawo landalama zomwe anthu akufuna kwabwino anapereka kwa Misita Ibu, Kuti ziwathandizire ku chipatala, atadwala kwa nthawi yayitali chakachatha. Kudwalaku kudachititsa kuti Misita. Ibu, adulidwe mwendo umodzi. | female | |
Malingana ndi akubanja kwake, katswiri wazisudzoyu, wachitidwaso ma operation asanu. Mneneri wanthambi yofufuza milandu mdzikolo. Maigan Aminati. | Malingana ndi akubanja kwake, katswiri wazisudzoyu, wachitidwaso ma opareshoni asanu. Mneneri wanthambi yofufuza milandu mdzikolo. Mayigani Aminati. | female | |
Wati akwanitsa kubwezeretsa ndalama zokwana 50,000,000, za mdziko la Nigeria. Malingana ndi Aminati, awiriwa anali ndi lingaliro lofuna kuthawira ku UK. | Wati akwanitsa kubwezeretsa ndalama zokwana fifite miliyoni, za mdziko la Nigeria. Malingana ndi Aminati, awiriwa anali ndi lingaliro lofuna kuthawira ku YUKE. | female | |
Atulutsidwa pa Bail la bwalo la milandu ndi chikole cha ndalama zokwana 15,000,000, zamdziko la Nigeria, pomwe kafukufuku pankhaniyi, akupitirira. | Atulutsidwa pa Belo la bwalo la milandu ndi chikole cha ndalama zokwana fifitini miliyoni, zamdziko la Nigeria, pomwe kafukufuku pankhaniyi, akupitirira. | female | |
Apolice amanga anthu awiri, omwe akuwaganizira kuti anaba katundu mugalimoto ya mu unduna wa zamtengatenga, yomwe imapita m’boma la Mwanza lachitatu. Malingana ndi mneneri wa a police mdzikomuno Peter Kalaya. | Apolisi amanga anthu awiri, omwe akuwaganizira kuti anaba katundu mugalimoto ya mu unduna wa zamtengatenga, yomwe imapita m’boma la Mwanza lachitatu. Malingana ndi mneneri wa a polisi mdzikomuno Pita Kalaya. | female | |
Awiriwa ndi a Alino Richard ndi Jonas Harold onse azaka 20, am’mudzi wa Lawundi mdera la mfumu Kanduku m’boma la Mwanza. | Awiriwa ndi a Lino Ritchadi ndi Jonasi Harodi onse azaka tuwente, am’mudzi wa Lawundi mdera la mfumu Kanduku m’boma la Mwanza. | female | |
Kalaya wati anthuwa ndi katundu yemwe anaba yemwe ndi Carpet komanso Tent akusungidwa pa police ya Mwanza. | Kalaya wati anthuwa ndi katundu yemwe anaba yemwe ndi kapeti komanso Tenti akusungidwa pa polisi ya Mwanza. | female | |
Anyamatawa anaba katunduyi mu galimoto ya mtundu wa Nissan Corona yomwe nambala yake ndi MG 476AL, pomwe imadutsa m’mudzi mwa Lawundi mu M6 wa Zalewa Mwanza. | Anyamatawa anaba katunduyi mu galimoto ya mtundu wa Nisani korona yomwe nambala yake ndi EMUJI folo sevevi sikisi e elo, pomwe imadutsa m’mudzi mwa Lawundi mu EMU sikisi wa Zalewa Mwanza. | female | |
Apolice amanga anthu awiri, omwe akuwaganizira kuti anaba katundu mugalimoto ya mu unduna wa zamtengatenga, yomwe imapita m’boma la Mwanza lachitatu. Malingana ndi mneneri wa a police mdzikomuno Peter Kalaya. | Apolisi amanga anthu awiri, omwe akuwaganizira kuti anaba katundu mugalimoto ya mu unduna wa zamtengatenga, yomwe imapita m’boma la Mwanza lachitatu. Malingana ndi mneneri wa a polisi mdzikomuno Pita Kalaya. | female | |
Unduna wazamalonda wapempha anthu ndi ma company ogulitsa nkhuku zamoyo kudzera m’magalimoto zoyendayenda mdzikomuno kuti apeze chiphaso chowayenereza kupanga malondawa ku undunawu ndicholinga chofuna kuti atukuke. | Unduna wazamalonda wapempha anthu ndi ma kampani ogulitsa nkhuku zamoyo kudzera m’magalimoto zoyendayenda mdzikomuno kuti apeze chiphaso chowayenereza kupanga malondawa ku undunawu ndicholinga chofuna kuti atukuke. | female | |
Mneneri mu undunawu Mayeso Msokera, wati undunawu upemphanso company zogulitsa nkhuku zikuluzikulu, kuti lizigulitsa nkhuku mopikulitsa chabe osati kuyendayenda m’madera. | Mneneri mu undunawu Mayeso Msokera, wati undunawu upemphanso kampani zogulitsa nkhuku zikuluzikulu, kuti lizigulitsa nkhuku mopikulitsa chabe osati kuyendayenda m’madera. | female | |
Ndicholinga choti anthu ndi ma company ang’onoang’ono ndi namene azichita izi kuti nawoso atukuke pachuma. Msokera wati undunawu ugwira ntchito limodzi ndi nthambi ya a police. | Ndicholinga choti anthu ndi ma kampani ang’onoang’ono ndi namene azichita izi kuti nawoso atukuke pachuma. Msokera wati undunawu ugwira ntchito limodzi ndi nthambi ya a polisi. | female | |
Komanso bungwe lolimbikitsa mpikisano ndi chilungamo pa malonda la Competitions and Trade Fair Commission CFTC, kuti malamulowa atsatiridwe mdzikomuno. | Komanso bungwe lolimbikitsa mpikisano ndi chilungamo pa malonda la kompitishonizi andi Thiredi Feya Komishoni (SI EFU TISI), kuti malamulowa atsatiridwe mdzikomuno. | female | |
Undunawu wati izi zadza, utawunikira kuti company zikuluzikulu zoweta nkhuku, zikuphangira ntchito zina zomwe ma company ang’onoang’ono amayenera kugwira, zomwe zikuchititsa kuti company zing’onozing’onozi, zilowe pansi. | Undunawu wati izi zadza, utawunikira kuti kampani zikuluzikulu zoweta nkhuku, zikuphangira ntchito zina zomwe ma kampani ang’onoang’ono amayenera kugwira, zomwe zikuchititsa kuti kampani zing’onozing’onozi, zilowe pansi. | female | |
Ku Nkhotakota, Ntchisi, Salima ndi maboma ena oyandikana ndi mabowa, Umunthu FM tsopano ikuveka pa 104.4 mega henz. | Ku Nkhotakota, Ntchisi, Salima ndi maboma ena oyandikana ndi mabowa, Umunthu EFU EMU tsopano ikuveka pa WANI ZIRO FOLO pointi folo mega henzi. | female | |
Pomwe ku Kasungu, Dowa, Ntcheu ndi maboma ena oyandikana ndi mabomawa, tikuveka pa 104.6 mega henz, muthaso kumvera kupsolera pa Internet kudzera pa Online Listening Link. | Pomwe ku Kasungu, Dowa, Ntcheu ndi maboma ena oyandikana ndi mabomawa, tikuveka pa WANI ZIRO FOLO pointi sikisi mega henzi, muthanso kumvera kupsolera pa Intaneti kudzera pa Onilayini Lisening'i Linki. | female | |
Mayi yemwe anabereka ana atatu pakamodzi, akufuna thandinzo. Mayiwa ndi a Madalitso zoto, azaka 24, am’mudzi wa Chipala mdera la mfumu Malengachanzi m’boma la Nkhotakota. | Mayi yemwe anabereka ana atatu pakamodzi, akufuna thandinzo. Mayiwa ndi a Madalitso zoto, azaka tuwente-folo, am’mudzi wa Chipala mdera la mfumu Malengachanzi m’boma la Nkhotakota. | female | |
Ndipo akupempha thandizo kwa anthu akufuna kwabwino, kuti akwanitse kusamalira ana awo atatu, omwe anabadwa pakamodzi. Madalitso watiuza kuti mamuna wake anamusiya ali ndi pathupi. | Ndipo akupempha thandizo kwa anthu akufuna kwabwino, kuti akwanitse kusamalira ana awo atatu, omwe anabadwa pakamodzi. Madalitso watiuza kuti mamuna wake anamusiya ali ndi pathupi. | female | |
Ndipo pakadalipano ali m’boma la Mangochi. Iye wati anawa atabadwa adamiyimbira lamya mamunayu, koma poyankha adati, eee! Koma ndiye chipsinjotu. | Ndipo pakadalipano ali m’boma la Mangochi. Iye wati anawa atabadwa adamiyimbira lamya mamunayu, koma poyankha adati, eee! Koma ndiye chipsinjotu. | female | |
Kuchokera pompo lamya ya mamunayu sigwira akayesera kuyimba, mayiyu wati akuvutika zedi kuti asamalire anawa, omwe anabadwa miyezi inayi yapitayo pa chipatala cha Saint Annie, m’bomali. | Kuchokera pompo lamya ya mamunayu sigwira akayesera kuyimba, mayiyu wati akuvutika zedi kuti asamalire anawa, omwe anabadwa miyezi inayi yapitayo pa chipatala cha Seyinti Anezi, m’bomali. | female | |
Pakadali pano, eni nyumba yomwe akukhala, akumuthamangitsa kamba koti wakhala miyezi yochuluka asakupereka ndalama ya nyumba. | Pakadali pano, eni nyumba yomwe akukhala, akumuthamangitsa kamba koti wakhala miyezi yochuluka asakupereka ndalama ya nyumba. | female | |
Mwazina iye wati akufuna thandizo la mkaka kuti anawa azimwa komanso thandizo la ndalalma kuti ayambirenso kuchita malonda a airtel money. | Mwazina iye wati akufuna thandizo la mkaka kuti anawa azimwa komanso thandizo la ndalalma kuti ayambirenso kuchita malonda a eyatelo maney. | female | |
Ponena kuti ali kale ndi ma card a agent, koma mwamunayo anawasiyitsa malondawa ali pa ubwenzi. Bungwe lowona za ntchito mphamva za magetsi la Malawi Energy Regulatory Authority MERA, | Ponena kuti ali kale ndi makadi a ejenti, koma mwamunayo anawasiyitsa malondawa ali pa ubwenzi. Bungwe lowona za ntchito mphamva za magetsi la Malawi Eneje Reguletare Osorite (MERA,) | female | |
Lati kukhazikika kwa mafuta a petrol mdziko muno, kwachepetsa mikangano pakati pa asodzi ndi ena m'malo omwetsera mafuta m'maboma a mphepete mwa nyanja. | Lati kukhazikika kwa mafuta a peturo mdziko muno, kwachepetsa mikangano pakati pa asodzi ndi ena m'malo omwetsera mafuta m'maboma a mphepete mwa nyanja. | female | |
Mneneri wa bungwe la MERA, Fitina Khonje, wauza Umunthu FM kuti kumapeto a chaka chatha, panali mikangano pomwe asodzi ena amadandaula kuti amakanizidwa kugula mafuta okagwiritsa ntchito ma bwato awo ophera nsomba | Mneneri wa bungwe la MERA, Fitina Khonje, wauza Umunthu EFU EMU kuti kumapeto a chaka chatha, panali mikangano pomwe asodzi ena amadandaula kuti amakanizidwa kugula mafuta okagwiritsa ntchito ma bwato awo ophera nsomba | female | |
Kaamba koti amasalidwa m'malowa. Khonje wati kukhazikika kwa mafuta a petrol mdziko muno kwapangitsa kuti mikanganoyi ithe kaamba koti asodziwa akumagula mafutawa munthawi yake. | Kaamba koti amasalidwa m'malowa. Khonje wati kukhazikika kwa mafuta a petrol mdziko muno kwapangitsa kuti mikanganoyi ithe kaamba koti asodziwa akumagula mafutawa munthawi yake. | female | |
iye wapempha asodziwa kuti ngati akupitilira kukumana ndi mavuto pogula mafutawa, azidziwitsa bungweli kuti lamulo ligwire ntchito. | iye wapempha asodziwa kuti ngati akupitilira kukumana ndi mavuto pogula mafutawa, azidziwitsa bungweli kuti lamulo ligwire ntchito. | female | |
Chaka chatha bungwe la MERA linakonza misankhano yophunzitsa asodzi komanso ochita malonda akuluakulu, kuti azidziwitsa bungweli ngati akukumana ndi mavuto pogula mafuta | Chaka chatha bungwe la MERA linakonza misankhano yophunzitsa asodzi komanso ochita malonda akuluakulu, kuti azidziwitsa bungweli ngati akukumana ndi mavuto pogula mafuta | female | |
komanso kuti apeze chiphaso chowaloleza kugula mafuta mosavuta. Chipani cha DPP chati sichodabwa kuona chipani cha MCP chikudandaula kamba koti chipani cha DPP chachotsa ena mwa mamembala ake mchipnichi. | komanso kuti apeze chiphaso chowaloleza kugula mafuta mosavuta. Chipani cha DIPIPI chati sichodabwa kuona chipani cha EMUSIPI chikudandaula kamba koti chipani cha DIPIPI chachotsa ena mwa mamembala ake mchipnichi. | female | |
kotero chayamba kuchita mantha kamba koti tsopano chipani cha DPP chabwelera mchimake. Namalomba wati ndizoseketsa kuona chipani cha MCP chili kakalikakali kuyankhula za chipani cha DPP | kotero chayamba kuchita mantha kamba koti tsopano chipani cha DiPiPi chabwelera mchimake. Namalomba wati ndizoseketsa kuona chipani cha EMUSIPI chili kakalikakali kuyankhula za chipani cha DiPiPi | female | |
Mmalo mokwaniritsa zomwe chidalonjeza amalawi chisanalowe mboma. Iye wati nacho chipani cha MCP mbuyomu chinachotsaponso mamembala ake koma chipani cha DPP chidakhala chete | Mmalo mokwaniritsa zomwe chidalonjeza amalawi chisanalowe mboma. Iye wati nacho chipani cha EMUSIPI mbuyomu chinachotsaponso mamembala ake koma chipani cha DIPIPI chidakhala chete | female | |
iye wati chipani cha MCP chili ndi mantha kamba koti nthawi yake yolamulira yatha kutsatira kuvutoka kwa amalawi ndipo ali ndi chikhulupiliro kuti chipani cha DPP chilowanso m'boma mchaka cha 2025 | iye wati chipani cha EMUSIPI chili ndi mantha kamba koti nthawi yake yolamulira yatha kutsatira kuvutoka kwa amalawi ndipo ali ndi chikhulupiliro kuti chipani cha DiPiPi chilowanso m'boma mchaka cha tuwente tuwente-fayifi | female | |
pakadalipano mlembi wa chipani cha MCP Ezekiel Ching'oma sanayankhulepo pa nkhaniyi. Katswiri pa nkhani za malamulo pa sukulu ya university of Malawi Dr. Benedete Malunga | pakadalipano mlembi wa chipani cha EMUSIPI Ezekiyelo Ching'oma sanayankhulepo pa nkhaniyi. Katswiri pa nkhani za malamulo pa sukulu ya Yunivesite ofu Malawi Dokota Benedete Malunga | female | |
wati udindo wa Kondwani Namkhumwa ngati mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma mnyumba ya malamulo, uli pa mpeni kutsatira kuchotsedwa kwake mu chipani cha Democratic Progressive (DPP) | wati udindo wa Kondwani Namkhumwa ngati mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma mnyumba ya malamulo, uli pa mpeni kutsatira kuchotsedwa kwake mu chipani cha Demokiratiki Purogiresivi (DiPiPi) | female | |
Malunga wati, lamulo limanena kuti munthu yemwe akuyenera kusankhidwa pa udundowo, ayenera kuchokera mu chipani chotsutsa boma chomwe chili ndi aphungu ochuluka mnyumba ya malamulo. | Malunga wati, lamulo limanena kuti munthu yemwe akuyenera kusankhidwa pa udundowo, ayenera kuchokera mu chipani chotsutsa boma chomwe chili ndi aphungu ochuluka mnyumba ya malamulo. | female | |
Malingana ndi Malunga, Namkhumwa akhoza kuchotsedwa pa udindowu, kamba koti adasankhidwa pa udindowu, nthawi yomwe adali membala wa chipani cha DPP | Malingana ndi Malunga, Namkhumwa akhoza kuchotsedwa pa udindowu, kamba koti adasankhidwa pa udindowu, nthawi yomwe adali membala wa chipani cha DIPIPI | female | |
kuchotsedwa kwa Namkhumwa ndi mammbala ena muchipani cha DPP, kunalengezedwa loweruka lapitrali. Anthu ena achipembedzo cha chisilamu apempha unduna wa zamaphunziro kuti ulingalirepo pankhani yokhala ndi maphunziro masana, | kuchotsedwa kwa Namkhumwa ndi mammbala ena muchipani cha DIPIP kunalengezedwa loweruka lapitrali. Anthu ena achipembedzo cha chisilamu apempha unduna wa zamaphunzilro kuti ulingalirepo pankhani yokhala ndi maphunziro masana, | female | |
Maka kwa ophunzira amu sukulu za pulayile, kamba koti izi zimakhuza maphunziro amadrasa, omwe ophunzira achipembedzochi amayenera kuphunzira | Maka kwa ophunzira amu sukulu za pulayile, kamba koti izi zimakhuza maphunziro amadirasa, omwe ophunzira achipembedzochi amayenera kuphunzira | female | |
Wachiwiri kwa mkhala pampando wa bungwe la Muslims Associations of Malawi, mboma la Salima, sheh Halun Chapola, anayankhula izi kumathero asabatayi | Wachiwiri kwa mkhala pampando wa bungwe la Muzilimuzi Asosiyeshoni ofu Malawi, mboma la Salima, shehi Haluni Chapola, anayankhula izi kumathero asabatayi | female | |
Pomwe a unduna wa zamaphunziro kudzera ku bungwe la Malawi insititute of Education amasonkhanitsa maganizo amalawi pazomwe zikuyenera kuyikidwa mundondomeka yatsopano ya maphunziro | Pomwe a unduna wa zamaphunziro kudzera ku bungwe la Malawi insitichuti ofu Ejukashoni amasonkhanitsa maganizo amalawi pazomwe zikuyenera kuyikidwa mundondomeka yatsopano ya maphunziro | female | |
poyamikira boma kamba kofikira mbali zokhuzidwa osiyanasiyana, kuphatikizapo atsogoleri a mipingo, Sheh Halun wapempha adindo kuti awunikire bwino maganizo omwe aperekedwa. | poyamikira boma kamba kofikira mbali zokhuzidwa osiyanasiyana, kuphatikizapo atsogoleri a mipingo, Shehi Haluni wapempha adindo kuti awunikire bwino maganizo omwe aperekedwa. | female | |
Ndicholinga choti maphunzira a mdziko muno apite patsogolo. Mmodzi mwa kholo yemwenso ndiwa chipembedzo cha chisilamu mboma la Salima, Yakubu Mussa, anadandaulanso za mikumano ina, | Ndicholinga choti maphunzira a mdziko muno apite patsogolo. Mmodzi mwa kholo yemwenso ndiwa chipembedzo cha chisilamu mboma la Salima, Yakubu Musa, anadandaulanso za mikumano ina, | female | |
yomwe sukulu zina zimakonza pa tsiku la chisau lomwe ndi tsiku lomwe anthu achipembedzo chisilamu amapemphera | yomwe sukulu zina zimakonza pa tsiku la chisau lomwe ndi tsiku lomwe anthu achipembedzo chisilamu amapemphera | female | |
Poyankhapo pa izi, mlembi mu unduna waza maphunziro Chikondano Musa, anatsimikizira amalawi kuti ndemanga zonse zomwe zatoleredwa, zikawunikiridwa bwino lomwe. | Poyankhapo pa izi, mlembi mu unduna waza maphunziro Chikondano Musa, anatsimikizira amalawi kuti ndemanga zonse zomwe zatoleredwa, zikawunikiridwa bwino lomwe. | female | |
Oyankhulapo pa nkhani za ndale akupitirira kuthirapo ndemanga pazomwe chipani cha MCP chachita, poyankhulapo pazomwe zikuchitika mu chipani cha DPP. | Oyankhulapo pa nkhani za ndale akupitirira kuthirapo ndemanga pazomwe chipani cha EMUSIPI chachita, poyankhulapo pazomwe zikuchitika mu chipani cha DiPiPi. | female | |
Victor chipofya wati, ngakhale palibe malamulo olesa chipani kuyankhulapo pazochitika za chipani china, komabe chipani cha MCP chikufuna kuoneka ngati chabwino kwa anthu omwe achotsedwa mu chipani cha DPP. | Vikita chipopfya wati, ngakhale palibe malamulo olesa chipani kuyankhulapo pazochitika za chipani china, komabe chipani cha EMUSIPI chikufuna kuoneka ngati chabwino kwa anthu omwe achotsedwa mu chipani cha cha DiPiPi. | female | |
Iye wati kuchotsedwa mchipani sizachilendo kamba koti izi zinachitikaponso pomwe chipani cha MCP chinachotsa a Jessy Kabwira komanso a Gostable Kaliwo ndi ena. | Iye wati kuchotsedwa mchipani sizachilendo kamba koti izi zinachitikaponso pomwe chipani cha EMUSIPI chinachotsa a Jese Kabwira komanso a Gositabo Kaliwo ndi ena. | female | |
Koma chipani cha DPP sichinayankhulepo kanthu pa izi, Chipofya ndiwodadwa kuti chifukwa chiyani chipani cha MCP chili kakalikakali ndi nkhani zochitika mchipani china, mmalo mothetsa mavuto omwe akuta dziko lino? | Koma chipani cha DiPiPi sichinayankhulepo kanthu pa izi, Chipofya ndiwodadwa kuti chifukwa chiyani chipani cha EMUSIPI chili kakalikakali ndi nkhani zochitika mchipani china, mmalo mothetsa mavuto omwe akuta dziko lino? | female | |
Pomwe Chipofya wati, palibe amayankhulapo za mnyumba mwa ena. chipani cha MCP chati, zimene zikuchitika mchipani cha DPP, nkusowa kulolerana. | Pomwe Chipofya wati, palibe amayankhulapo za mnyumba mwa ena. chipani cha EMUSIPI chati, zimene zikuchitika mchipani cha DiPiPi, nkusowa kulolerana. | female | |
Oyankhulapo pa nkhani za ndale clement Makuwa, sakuona kulakwitsa kulikonse pazomwe chipani cha MCP chachita poyankhulapo pazomwe zikuchitika mchipani cha DPP. | Oyankhulapo pa nkhani za ndale kilementi Makuwa, sakuona kulakwitsa kulikonse pazomwe chipani cha EMUSIPI chachita poyankhulapo pazomwe zikuchitika mchipani cha DiPiPi. | female | |
Chipani cha MCP chadzudzula kuchotsedwa kwa mamembala ena mchipani cha DPP ponene kuti izi zikuonetsa kuti mchipanichi mulibe kulolerana. | Chipani cha EMUSIPI chadzudzula kuchotsedwa kwa mamembala ena mchipani cha DiPiPi ponene kuti izi zikuonetsa kuti mchipanichi mulibe kulolerana. | female | |
Ena akuona kuti, zomwe chachita chipani cha MCP, zikuonetsa ngati kuti, ndichomwe chimatuma ena mwa mamembala a DPP, kuti azidzetsa chisokonezo mchipani chawo | Ena akuona kuti, zomwe chachita chipani cha EMUSIPI, zikuonetsa ngati kuti, ndichomwe chimatuma ena mwa mamembala a DiPiPi, kuti azidzetsa chisokonezo mchipani chawo | female | |
koma Makuwa wati zomwe chipani cha DPP chachita, zili mkamwamkamwa mwa aliyense mdziko muno, ndipo aliyense kuphatikizapo zipani zina zandale, zitha kuthirirapo ndemanga pa izi. | koma Makuwa wati zomwe chipani cha DPP chachita, zili mkamwamkamwa mwa aliyense mdziko muno, ndipo aliyense kuphatikizapo zipani zina zandale, zitha kuthirirapo ndemanga pa izi. | female | |
Makuwa watsindika kunena kuti, ndikwabwino kulolerana ndikulimbikitsa umodzi mchipani pa nthawi yomwe pali kusemphana zochita. | Makuwa watsindika kunena kuti, ndikwabwino kulolerana ndikulimbikitsa umodzi mchipani pa nthawi yomwe pali kusemphana zochita. | female | |
Chipani cha MCP chadzudzula kuchotsedwa kwa mamembala ena mchipani cha DPP, ponene kuti izi nzotsutsana ndi ulamuliro wa demokalase | Chipani cha EMUSIPI chadzudzula kuchotsedwa kwa mamembala ena mchipani cha DiPiPi ponene kuti izi nzotsutsana ndi ulamuliro wa demokalase | female | |
Kudzera kwa mlembi wake Ezekiel Ching'oma, chipani cha MCP chati nzodandaulitsa kuti chipani cha DPP chikuchita zinthu zosemphana ndi msanamila za ulamuliuro wa demokalase zome chipanichi chinakhazikitsidwira | Kudzera kwa mlembi wake Ezekiel Ching'oma, chipani cha EMUSIPI chati nzodandaulitsa kuti chipani cha DiPiPi chikuchita zinthu zosemphana ndi msanamila za ulamuliuro wa demokalase zome chipanichi chinakhazikitsidwira | female | |
Apa chipani cha MCP chapempha chipani cha DPP kuti chiganizire zosintha ganizo lochotsa mchipanichi, ena mwa mamembala ake. | Apa chipani cha EMUSIPI chapempha chipani cha DiPiPi kuti chiganizire zosintha ganizo lochotsa mchipanichi, ena mwa mamembala ake. | female | |
nkuchita zinthu ngati momwe zipani zina zikuchitira, maka polola kumva maganizo a ena, Loweruka lapitali a Kondwani Namkhumwa, Grizeder Jefrey, Nicolus Dausi mwa ena, achotsedwa mchipanichi. | nkuchita zinthu ngati momwe zipani zina zikuchitira, maka polola kumva maganizo a ena, Loweruka lapitali a Kondwani Namkhumwa, Girizeda Jefure, Nikolasi Dausi mwa ena, achotsedwa mchipanichi. | female | |
Chipani cha DPP chati, anthuwa amachita zinthu zosemphana ndi malamulo achipanichi, chipani cha DPP chachotsa mchipanichi ena mwa mamembala ake monga Kondwani Namkhumwa, Grizeder Jefrey, | Chipani cha DiPiPi chati, anthuwa amachita zinthu zosemphana ndi malamulo achipanichi, chipani cha DiPiPi chachotsa mchipanichi ena mwa mamembala ake monga Kondwani Namkhumwa, Girizeda Jefure, | female | |
Cicilia Chadzama, Nicolus Dausi ndi Mark Botomani. Chikalata chomwe chasayiniridwa ndi mneneri wachipanichi, Shadreck Namalomba, | Sisiliya Chadzama, Nikolasi Dausi ndi Maki Botomani. Chikalata chomwe chasayiniridwa ndi mneneri wachipanichi, Shadireki Namalomba, | female | |
chati ganizoli ladza kutsatira mkumano wa committee yayikulu ya chipanichi omwe unaliko lero. Ena mwa omwe achotsedwa ndi Otria Jere, Fortunate Semion Phiri, Fredrick Billy Malata, | chati ganizoli ladza kutsatira mkumano wa komiti yayikulu ya chipanichi omwe unaliko lero. Ena mwa omwe achotsedwa ndi Otiriya Jere, Fochuneti Simiyoni Phiri, Furediriki Bile Malata, | female | |
Joe Thomas Nyirongo ndi Keneth Chatata Nsonda. mamembalawa anakawonekere ku komiti yosungitsa mwambo mchipanichi posachedwapa kamba kotsogolera ndi kukhalanawo pa mkumano wa akuluakulu a chipanichi, | Jo Thomasi Nyirongo ndi Kenefi Chatata Nsonda. mamembalawa anakawonekere ku komiti yosungitsa mwambo mchipanichi posachedwapa kamba kotsogolera ndi kukhalanawo pa mkumano wa akuluakulu a chipanichi, | female | |
Womwe unachitika pa 6 Disembala, chaka chatha mu mzinda wa Lilongwe. Pakadalipano chipanichi chalimbikitsa mamembala ake kuti akuyenera kutsatira izi. | Womwe unachitika pa sikisi Disembala, chaka chatha mu mzinda wa Lilongwe. Pakadalipano chipanichi chalimbikitsa mamembala ake kuti akuyenera kutsatira izi. | female | |
Bungwe lomwe limamenyera ufulu a anthu othawa kwawo lotchedwa INUWA Advocacy, lawuza anthu othawa kwawo omwe ali mdziko muno, kuti azikaneneza kwa adindo oyenerera akachitiridwa nkhanza ndi azachitetezo. | Bungwe lomwe limamenyera ufulu a anthu othawa kwawo lotchedwa INUWA Adivokase, lawuza anthu othawa kwawo omwe ali mdziko muno, kuti azikaneneza kwa adindo oyenerera akachitiridwa nkhanza ndi azachitetezo. | female | |
Mawuwa akudza kusatira zomwe bwanamkubwa wa khonsolo ya mzinda wa Lilongwe, Dr. Lawful Palani wanena kuti anthu onse othawa kwawo omwe abwereranso mu mzindawu, | Mawuwa akudza kusatira zomwe bwanamkubwa wa khonsolo ya mzinda wa Lilongwe, Dokota Lofuu Palani wanena kuti anthu onse othawa kwawo omwe abwereranso mu mzindawu, | female | |
abwere kumalo osungira anthu othawa kwawo a dzaleka mboma la Dowa msanga. Mmodzi wa akuluakulu ku bungweli, Matchona Phiri, | abwere kumalo osungira anthu othawa kwawo a dzaleka mboma la Dowa msanga. Mmodzi wa akuluakulu ku bungweli, Matchona Phiri, | female | |
Wati anthuwa amapita mzindawu kuti akatenge katundu ndi ndalama zawo, osati kuphwanya malamulo. Iye wati omwe anataya ndalama komanso katundu pantchito yowabwezeretsa ku dzaleka akukhala movutika. | Wati anthuwa amapita mzindawu kuti akatenge katundu ndi ndalama zawo, osati kuphwanya malamulo. Iye wati omwe anataya ndalama komanso katundu pantchito yowabwezeretsa ku dzaleka akukhala movutika. | female | |
kamba koti akukanika kuti ayambirenso kukhala moyo watsopano. Apolice m'boma la Nkhotakota amanga Steve Manda wa zaka 34 kamba koziyerekeza ngati ntsirikali. | kamba koti akukanika kuti ayambirenso kukhala moyo watsopano. Apolisi m'boma la Nkhotakota amanga Sitivi Manda wa zaka sete-folo kamba koziyerekeza ngati ntsirikali. | female | |
ndikumatenga ndalama komanso mowa kwa anthu pa nsika wapa boma m'bomali, powalamula kuti ali ndi mphamvu zochitira izi. Wachiwiri kwa mneneri wa police ya Nkhotakota, Chisomo Chuma, | ndikumatenga ndalama komanso mowa kwa anthu pa nsika wapa boma m'bomali, powalamula kuti ali ndi mphamvu zochitira izi. Wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Nkhotakota, Chisomo Chuma, | female | |
wati anthu ena anadabwa ndi khalidweli, ndipo anatsina khutu apolice. Kutsatira izi a Police anamanga bamboyo, ndikumupititsa ku police ya Nkhotakota, kuti akafotoze bwino za izi. | wati anthu ena anadabwa ndi khalidweli, ndipo anatsina khutu apolisi. Kutsatira izi a Polisi anamanga bamboyo, ndikumupititsa ku polisi ya Nkhotakota, kuti akafotoze bwino za izi. | female | |
ku polisiku iye anavomereza kuti amachita khalidweli komanso kuti sagwira ntchito ku nthambi ya chitetezo yatsirikali, kenako anamumanga. | ku polisiku iye anavomereza kuti amachita khalidweli komanso kuti sagwira ntchito ku nthambi ya chitetezo yatsirikali, kenako anamumanga. | female | |
Steve yemwe ndiwa mmudzi mwa mwamulowe mboma la Rumphi, akawonekera ku bwalo la mlandu posachedwapa kukayankha mlandu woziyerekeza ngati wachitetezo. | Sitivi yemwe ndiwa mmudzi mwa mwamulowe mboma la Rumphi, akawonekera ku bwalo la mlandu posachedwapa kukayankha mlandu woziyerekeza ngati wachitetezo. | female | |
Office ya zaulimi ya m'boma la Nkhotakota yati ndiyokhutira ndi momwe ntchito yopereka zipangizo zaulimi zotsika mtengo zikuyendera m'bomali. Mkulu wa zamalimidwe m'bomali Firiyo Nkhukuzalira Magomero, | Ofesi ya zaulimi ya m'boma la Nkhotakota yati ndiyokhutira ndi momwe ntchito yopereka zipangizo zaulimi zotsika mtengo zikuyendera m'bomali. Mkulu wa zamalimidwe m'bomali Firiyo Nkhukuzalira Magomero, | female | |
wauza umunthu FM kuti pofika lolemba sabata ino, pa anthu 40,754 omwe akupindula ndi zipangizo zaulimi zotsika mtengozi, anthu 94 pa 100 aliwonse, | wauza umunthu EFU EMU kuti pofika lolemba sabata ino, pa anthu fote sauzandi seveni handiuredi andi fifite-folo omwe akupindula ndi zipangizo zaulimi zotsika mtengozi, anthu nayinte-folo pa wani handiredi aliwonse, | female | |
ndiwo akwanaitsa kugula feteleza wanthaka ndipo anthu 60 pa 100 aliwonse ndiwomwe agula feteleza wobereketsa. Magomwero wati izi zathekakamba ka mgwirizano wa pakati pa office yawo | ndiwo akwanaitsa kugula feteleza wanthaka ndipo anthu sikisite pa wani handiredi aliwonse ndiwomwe agula feteleza wobereketsa. Magomwero wati izi zathekakamba ka mgwirizano wa pakati pa ofesi yawo | female | |
ndi adindo ena omwe anatengapo mbali kuthandizira kuti zipangizozi zifike madera ena omwe amavuta mayendedwe monga kwa Mwansambo komanso kulupashi munthawi yoyenera. | ndi adindo ena omwe anatengapo mbali kuthandizira kuti zipangizozi zifike madera ena omwe amavuta mayendedwe monga kwa Mwansambo komanso kulupashi munthawi yoyenera. | femalo | |
Iye anawonjezera kunena kuti mwa anthu 620 omwe analembedwa mu kaundula wa anthu opindula ndi zipangizozi kudera la Lupashi, anthu 610 akwanitsa kugula feteleza yense wofunika komanso mbewu. | Iye anawonjezera kunena kuti mwa anthu sikisi handiredi andi tuwente omwe analembedwa mu kaundula wa anthu opindula ndi zipangizozi kudera la Lupashi, anthu sikisi handiredi andi teni akwanitsa kugula feteleza yense wofunika komanso mbewu. | female | |
Kampani yopanga magetsi mdziko muno ya Electricty Generation Company (Egenco) yati yatsirizitsa ntchito yokonzanso malo opangira magetsi a Mkula B | Kampani yopanga magetsi mdziko muno ya Elekitirisite Jenereshoni Kampani (Ejenko) yati yatsirizitsa ntchito yokonzanso malo opangira magetsi a Mkula Bi | female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.