audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
usiku wa lamulungu. zomwe zachititsa kuti magetsi abwererenso mchimake. mneneri wa kampaniyi, Moses Gwaza, wauza Umunthu EFU EMU | usiku wa lamulungu. zomwe zachititsa kuti magetsi abwererenso mchimake. mneneri wa kampaniyi, Mozesi Gwaza, wauza Umunthu FM | female | |
kuti ntchito yofufuza chomwe chinavuta pamalowa, inapeza kuti mkati mwa pipe ina yolowetsera madzi munali tsinde la mtengo, zinthu zomwe zinachititsa kuti makina ena asagwire ntchito bwino. | kuti ntchito yofufuza chomwe chinavuta pamalowa, inapeza kuti mkati mwa payipi ina yolowetsera madzi munali tsinde la mtengo, zinthu zomwe zinachititsa kuti makina ena asagwire ntchito bwino. | femalo | |
Pakadalipano Gwaza wati, kampaniyi yakhazikitsa ndondomeko zosiyanasiyana, zowonetsetsa kuti magetsi azipezeka pomwe nyengo ya mvula yayamba. | Pakadalipano Gwaza wati, kampaniyi yakhazikitsa ndondomeko zosiyanasiyana, zowonetsetsa kuti magetsi azipezeka pomwe nyengo ya mvula yayamba. | female | |
koma iye sanabise mawu kuti pomwe nyengo ya mvula yayamba, kuzimazima kwa magetsi kuzikhalapo ndithu kamba ka ngozi zodza chifukwa cha mvula | koma iye sanabise mawu kuti pomwe nyengo ya mvula yayamba, kuzimazima kwa magetsi kuzikhalapo ndithu kamba ka ngozi zodza chifukwa cha mvula | female | |
Kuchokera loweruka lapitali, pafupifupi maboma onse mdziko muno akumana ndi vuto lakuthimathima kwa magetsi. Akukaseweza ndende kamba kotchola nkhungudzu mwa mnyamata wa chisidzera. | Kuchokera loweruka lapitali, pafupifupi maboma onse mdziko muno akumana ndi vuto lakuthimathima kwa magetsi. Akukaseweza ndende kamba kotchola nkhungudzu mwa mnyamata wa chisidzera. | female | |
Mzimayi wina wa mboma la kasungu wa zaka zakubadwa 38, Takondwa Banda, chaka chino chikhala chosayiwalika mmoyo mwake pomwe wagamulidwa kukakhala kundende kwa zaka khumi zisanu ndi chimodzi (16), | Mzimayi wina wa mboma la kasungu wa zaka zakubadwa sete-eyiti, Takondwa Banda, chaka chino chikhala chosayiwalika mmoyo mwake pomwe wagamulidwa kukakhala kundende kwa zaka khumi zisanu ndi chimodzi (sikisitini), | female | |
atapezeka wolakwa pa mlandu wochita zachisembwere ndi mnyamata wa nthete wa zaka 16 zakubadwa. Wofalitsa nkhani za police ku Kasungu Joseph Kachikho, | tapezeka wolakwa pa mlandu wochita zachisembwere ndi mnyamata wa nthete wa zaka sikisitini zakubadwa. Wofalitsa nkhani za polisi ku Kasungu Jozefe Kachikho, | female | |
wati woyimira boma pa milandu, Martha Mwenechanya, anauza bwaloli kuti mayiyu anapalamula mlanduwu usiku wina, pomwe anamukokera mnyamatayo kuchipinda kwake nkuyamba kumuonetsa kanema wolawula, | wati woyimira boma pa milandu, Mafa Mwenechanya, anauza bwaloli kuti mayiyu anapalamula mlanduwu usiku wina, pomwe anamukokera mnyamatayo kuchipinda kwake nkuyamba kumuonetsa kanema wolawula, | female | |
kenaka pamapeto pa zonse anagona naye. posakhutitsidwabe ndi izi, tsiku lina mayiyo anakokeranso mnyamatayo pa tchire, | kenaka pamapeto pa zonse anagona naye. posakhutitsidwabe ndi izi, tsiku lina mayiyo anakokeranso mnyamatayo pa tchire, | female | |
nkugonanayenso ndipo apa ndipomwe mnyamatayo anaganiza zokanena kwa mayi ake omwe anakatula nkhaniyi ku police. Banda amachokera ku m'mudzi mwa Misi mboma lomwelo la Kasungu | nkugonanayenso ndipo apa ndipomwe mnyamatayo anaganiza zokanena kwa mayi ake omwe anakatula nkhaniyi ku police. Banda amachokera ku m'mudzi mwa Misi mboma lomwelo la Kasungu | female | |
Nthambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya Department of disaster and management affairs, yati maboma okwana khumi ndi anayi mdziko muno, ndi omwe akhuzidwa kamba ka ngozi zoyiyanasiyana | Nthambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzidzi ya Dipatimenti ofu dizasita andi manejimenti afeyazi, yati maboma okwana khumi ndi anayi mdziko muno, ndi omwe akhuzidwa kamba ka ngozi zoyiyanasiyana | female | |
chiyambireni nyengo ya mvula chaka chino. Malingana ndi chikalata chomwe nthambiyi yatulutsa lachinayi, ngozizi ndi monga ziphaliwali, mphepo ya mkuntho komanso mvula ya mphamvu yodza ndi mphepo mwa zina. | chiyambireni nyengo ya mvula chaka chino. Malingana ndi chikalata chomwe nthambiyi yatulutsa lachinayi, ngozizi ndi monga ziphaliwali, mphepo ya mkuntho komanso mvula ya mphamvu yodza ndi mphepo mwa zina. | female | |
Nthambiyi yati chiwerengero cha anthu omwe akhudzidwa pakadalipano chakwera kuchoka 961 kufika pa 4751. | Nthambiyi yati chiwerengero cha anthu omwe akhudzidwa pakadalipano chakwera kuchoka nayini handiredi andi sikisite-wani kufika pa folo sauzandi seveni handiredi andi fifite-wani. | female | |
Ndipo mwachiwerengerochi anthu asanu afa atawombedwa ndi mphezi pomwe anthu 46 avulala mosiyanasiyana. | Ndipo mwachiwerengerochi anthu asanu afa atawombedwa ndi mphezi pomwe anthu fote-sikisi avulala mosiyanasiyana. | female | |
Bungwe lolembetsa mayeso mdziko muno la Malawi National Examinations Board (MANEB), lati sipakhalanso kuwonjezera nthawi kulikonse kwa ophunzira omwe akuyenera kuperaka ndalama yolembera mayeso. | Bungwe lolembetsa mayeso mdziko muno la Malawi Neshono Egizamineshonzi Boodi (MANEBU), lati sipakhalanso kuwonjezera nthawi kulikonse kwa ophunzira omwe akuyenera kuperaka ndalama yolembera mayeso. | female | |
Mkulu wa bungweli Dolothy Nampota wati bungweli pakadalipano lili pa mpanipani pofuna kuyamba ntchito yopanga mapepala amayeso, ndipo palibenso zoonjezera nthawi iliyonse | Mkulu wa bungweli Dolofe Nampota wati bungweli pakadalipano lili pa mpanipani pofuna kuyamba ntchito yopanga mapepala amayeso, ndipo palibenso zoonjezera nthawi iliyonse | female | |
Tawonjezera nthawi mokwanira, ndipo izi zatiyikanso pampanipani. Chifukwa tikuthamangira nthawi yopanga mapepala amayeso, kuwonjera nthawi kwathera pompa basi. Watero Nampota. | Tawonjezera nthawi mokwanira, ndipo izi zatiyikanso pampanipani. Chifukwa tikuthamangira nthawi yopanga mapepala amayeso, kuwonjera nthawi kwathera pompa basi. Watero Nampota. | female | |
Koma pakadalipano oyankhulapo pankhani za maphunziro, Victor Chikoti, wati nthawi yomwe bungwe la MANEB yawonjezera ndiyochepa kwambiri, potengera kuti ophunzira ambiri akulepherabe kupereka ndalama ya mayeso. | Koma pakadalipano oyankhulapo pankhani za maphunziro, Vikita Chikoti, wati nthawi yomwe bungwe la MANEBu yawonjezera ndiyochepa kwambiri, potengera kuti ophunzira ambiri akulepherabe kupereka ndalama ya mayeso. | female | |
Bungwe la MANEB lalengeza kuti lawonjezera nthawi yomwe ophunzira akuyenera kulipira ndalama ya mayeso a standard 8, form 2 komanso form 4, | Bungwe la MANEBU lalengeza kuti lawonjezera nthawi yomwe ophunzira akuyenera kulipira ndalama ya mayeso a sitandade eyiti, fomu thu komanso fomu folo, | female | |
kuchokera pa 8 kufika pa 12 January, 2024, ophunzira pafupifupi 29 000 ndiwomwe pakadalipano sanaperekebe ndalama yawo ya mayeso, zinthu zomwe zikuyika chiwopsezo ngati angalembenawo mayeso. | kuchokera pa eyiti kufika pa thuwelofu Januware, tuwente tuwente-folo, ophunzira pafupifupi tuwente-nayini sauzandi ndiwomwe pakadalipano sanaperekebe ndalama yawo ya mayeso, zinthu zomwe zikuyika chiwopsezo ngati angalembenawo mayeso. | female | |
Mnyamata wina wa zaka 29 boma la Kasungu Greatness Juma, wakhala akumangidwa pa chain kwa chaka tsopano kamba kavuto lamaganizo angwiro. | Mnyamata wina wa zaka tuwente nayini boma la Kasungu Giretinesi Juma, wakhala akumangidwa pa tcheni kwa chaka tsopano kamba kavuto lamaganizo angwiro. | female | |
Mayi ake a mnyamatayu Lizie Juma, ati vutoli linayamba mchaka cha 2016, ndipo ayesetsa kuyenda muzipatala zosiyanasiyana kuphatikizapo chipatala chothandiza anthu avutoli cha Zomba, koma izi sizinaphule kanthu. | Mayi ake a mnyamatayu Lizi Juma, ati vutoli linayamba mchaka cha tuwente sikisitini, ndipo ayesetsa kuyenda muzipatala zosiyanasiyana kuphatikizapo chipatala chothandiza anthu avutoli cha Zomba, koma izi sizinaphule kanthu. | femalo | |
Madotolo kumeneko amati mnyamatayu alibe vuto la maganizo angwiro. Mayiwa ati vutoli lafikapo Greatiness amachita zinthu zosokoneza monga kuwamenya, kuima pakati pa msewu wawukulu wa M1 komanso kuphwanya katundu. | Madotolo kumeneko amati mnyamatayu alibe vuto la maganizo angwiro. Mayiwa ati vutoli lafikapo Giretinesi amachita zinthu zosokoneza monga kuwamenya, kuima pakati pa msewu wawukulu wa EME wani komanso kuphwanya katundu. | female | |
Zinthu zomwe zinachititsa kuganiza kuti azimumangirira pamtengo ndi Chain. Pomwe Umunthu FM, inapita kukamuona Greatness, tinampeza ali ndi bala pa mwendo wamazere. Iye wati anthu ena anachita chomumenya ndi chitsulo. | Zinthu zomwe zinachititsa kuganiza kuti azimumangirira pamtengo ndi Cheni. Pomwe Umunthu EFU EMU, inapita kukamuona Giretinesi, tinampeza ali ndi bala pa mwendo wamazere. Iye wati anthu ena anachita chomumenya ndi chitsulo. | female | |
Mayi ake atsimikizanso za izi. Mfumu Chibwira, yomwe imakhala moyandikana ndi kwawo kwa mnyamatayu, yati vutoli likafikapo, amatha kuwavulaza mayi ake. | Mayi ake atsimikizanso za izi. Mfumu Chibwira, yomwe imakhala moyandikana ndi kwawo kwa mnyamatayu, yati vutoli likafikapo, amatha kuwavulaza mayi ake. | female | |
Mfumuyi, yapempha anthu akufuna kwabwino, kuti awathandize mayiwa, poti njira zonse zomwe atsata, sizinaphule kanthu. | Mfumuyi, yapempha anthu akufuna kwabwino, kuti awathandize mayiwa, poti njira zonse zomwe atsata, sizinaphule kanthu. | female | |
Katswiri wochita masewero othamanga wadziko la South Africa, koma yemwe ali olumala ndipo anadulidwa miyendo yonse, Oscar Pistorious, tsopano amukhululukira kuti atuluke kundende. | Katswiri wochita masewero othamanga wadziko la Sowufi Afirika, koma yemwe ali olumala ndipo anadulidwa miyendo yonse, Osika Pisitoriyasi, tsopano amukhululukira kuti atuluke kundende. | female | |
Pistorious yemwe adamangidwa zaka khumi ndi chimodzi zapitazo, 11, pamulandu wopezeka olakwa atapha bwenzi lake poliwombera ndi mfuti, wakhululukiridwa atagwira theka la ukayidi wazaka zomwe anagamulidwa kuti akaseweze ku jere. | Pisitoriyasi yemwe adamangidwa zaka khumi ndi chimodzi zapitazo, leveni, pamulandu wopezeka olakwa atapha bwenzi lake poliwombera ndi mfuti, wakhululukiridwa atagwira theka la ukayidi wazaka zomwe anagamulidwa kuti akaseweze ku jere. | female | |
Akuluakulu a ndende yomwe iye anali, atsimikizira nyumba yowulutsa mawu ya BBC, kuti pofika lachisanu, katswiri wothamangayu, anali atafika kale kunyumba yake. | Akuluakulu a ndende yomwe iye anali, atsimikizira nyumba yowulutsa mawu ya BIBISI, kuti pofika lachisanu, katswiri wothamangayu, anali atafika kale kunyumba yake. | female | |
Pistorious yemwe tsopano ali ndi zaka 37, adawombera bwenzi lakero kangapo muchaka cha 2013, kudzera pakhomo. Pambuyo pake mkuluyu adawuza bwalo lamilandu, kuti adamuyesa bwezi wakeyo ngati wakuba. | Pisitoriyasi yemwe tsopano ali ndi zaka 3sete seveni, adawombera bwenzi lakero kangapo muchaka cha tuwente setini, kudzera pakhomo. Pambuyo pake mkuluyu adawuza bwalo lamilandu, kuti adamuyesa bwezi wakeyo ngati wakuba. | female | |
Pistorious, adapezeka ndi mulandu wakupha mu 2015, pomwe court la appeal lidathetsa chigamulo choyambirira cha kupha munthu mwadala. | Pisitoriyasi, adapezeka ndi mulandu wakupha mu tuwente fifitini, pomwe khoti la apilo lidathetsa chigamulo choyambirira cha kupha munthu mwadala. | female | |
Pansi pa malamulo a dziko la South Africa, olakwa onse ali ndi ufulu, woganiziridwa kuti atha kukhululukiridwa, akamaliza theka la chilango chawo chonse. | Pansi pa malamulo a dziko la Sowufi Afirika, olakwa onse ali ndi ufulu, woganiziridwa kuti atha kukhululukiridwa, akamaliza theka la chilango chawo chonse. | female | |
Inde atikwenzera malipiro, komabe timayembekeza ndalama yokwererapo. Mkulu wabungwe lowona za anthu ogwira ntchito mdzikomuno la Malawi Congress of Trade Union, MCTU. Charles Kumchenga. | Inde atikwenzera malipiro, komabe timayembekeza ndalama yokwererapo. Mkulu wabungwe lowona za anthu ogwira ntchito mdzikomuno la Malawi kongiresi ofu Thiredi Yuniyoni, (EMUSITIYU). Tchalosi Kumchenga. | female | |
Wati boma lachita bwino kukweza ndalama ya anthu ogwira ntchito m’boma, komabe wadandawula kuti ndalamayi ndiyochepa. | Wati boma lachita bwino kukweza ndalama ya anthu ogwira ntchito m’boma, komabe wadandawula kuti ndalamayi ndiyochepa. | female | |
Iye wawuza Umunthu fm, kuti kukwezedwa kwa ndalamayi, komwe kwawonjenzeredwa ndi 15 kwacha pa 100 kwacha iliyonse yomwe munthu amalandira, nkosapindulitsa kwenikweni. | Iye wawuza Umunthu EFU EMU, kuti kukwezedwa kwa ndalamayi, komwe kwawonjenzeredwa ndi fifitini kwacha pa wani handiredi kwacha iliyonse yomwe munthu amalandira, nkosapindulitsa kwenikweni. | female | |
Ndalamayi yakwezedwa inde, tavomereza mwachoncho, komano timayembekezera kuti boma likweza mopitirira mulingo womwe wayikidwawu, komabe tikungodikira mwezi wa Malichi chaka chomwechino. | Ndalamayi yakwezedwa inde, tavomereza mwachoncho, komano timayembekezera kuti boma likweza mopitirira mulingo womwe wayikidwawu, komabe tikungodikira mwezi wa Malichi chaka chomwechino. | female | |
Pomwenso tikhale ndi zokambirana ndi mbali yaboma, pofuna kuwona ngati ndalamayi ingakwedwebe. Watero Kumchenga. Chaka chatha boma lidalengeza za lingaliro lake lofuna kukweza ndalama yomwe anthu ogwira ntchito m’boma amalandira. | Pomwenso tikhale ndi zokambirana ndi mbali yaboma, pofuna kuwona ngati ndalamayi ingakwedwebe. Watero Kumchenga. Chaka chatha boma lidalengeza za lingaliro lake lofuna kukweza ndalama yomwe anthu ogwira ntchito m’boma amalandira. | female | |
Ndi 10 kwacha pa 100 kwacha iliyonse, kutsatira kutsika mphavu kwandalama ya kwacha, koma izi anthu ambiri adanyinyirika nazo. | Ndi teni kwacha pa wani handiredi kwacha iliyonse, kutsatira kutsika mphavu kwandalama ya kwacha, koma izi anthu ambiri adanyinyirika nazo. | female | |
Yemwe amalankhulapo pa nkhani za achinyamata mdzikomuno, Lucky Mbewe, wapempha achinyamata kuti apewe kugwiritsidwa ntchito ndi anthu andale, pomwe dzikolino, likhale likuchititsa zisankho mchaka cha 2025. | Yemwe amalankhulapo pa nkhani za achinyamata mdzikomuno, Lake Mbewe, wapempha achinyamata kuti apewe kugwiritsidwa ntchito ndi anthu andale, pomwe dzikolino, likhale likuchititsa zisankho mchaka cha tuwente tuwente-fayifi. | female | |
Mbewe wati achinyamata akuyenera kupewa mchitidwewu, kamba koti nthawi zambiri, anthu andale amawasambira m’manja akakumana ndi mavuito monga kumangidwa ndi zina, pomwe iwo amakhala akukondwera m’makomo mwawo. | Mbewe wati achinyamata akuyenera kupewa mchitidwewu, kamba koti nthawi zambiri, anthu andale amawasambira m’manja akakumana ndi mavuito monga kumangidwa ndi zina, pomwe iwo amakhala akukondwera m’makomo mwawo. | female | |
Iye wawonjenzera kuti ngakhale kusowa kwa ntchito kuli chida chimodzi chomwe chikuchititsa kuti andale azigwiritsa ntchito achinyamata, monga kuyambitsa zipolowe nthawi ya misonkhano yokopa anthu, | Iye wawonjenzera kuti ngakhale kusowa kwa ntchito kuli chida chimodzi chomwe chikuchititsa kuti andale azigwiritsa ntchito achinyamata, monga kuyambitsa zipolowe nthawi ya misonkhano yokopa anthu, | female | |
Achinyamata akuyenera kudzidalira pawokha,komaso kukhala wochenjera kumchitidwewoterewu. Mwana wazaka 10, dalayivala, komanso wothandizira dalayivala, | Achinyamata akuyenera kudzidalira pawokha,komaso kukhala wochenjera kumchitidwewoterewu. Mwana wazaka teni, dalayivala, komanso wothandizira dalayivala, | female | |
Afa pangozi yagalimoto, mdera la Kapala ku Dwangwa, m’boma la Nkhotakota. Ngoziyi yachitika pa 14 mwezi uno, ndipo yakhudza galimoto ya mtundu wa Toyota Sienta. | Afa pangozi yagalimoto, mdera la Kapala ku Dwangwa, m’boma la Nkhotakota. Ngoziyi yachitika pa fotini mwezi uno, ndipo yakhudza galimoto ya mtundu wa Toyota Siyenta. | female | |
Yomwe number yake ndi CP6433, ndipo yinanyamula anthu asanu ndi atatu, (8). Malingana ndi mneneri wa police ya Nkhunga m’bomali. Andrew Kamanga. | Yomwe nambala yake ndi SIPI sikisi folo firfiri, ndipo yinanyamula anthu asanu ndi atatu, (eyiti). Malingana ndi mneneri wa polisi ya Nkhunga m’bomali. Anduru Kamanga. | female | |
Patsikuli driver wagalimotoli, Aaron Simenti, amafuna kudutsa galimoto yomwe sikudziwika, koma analephera kuwongolera bwino galimotolo, kamba kothamangitsa kwambiri, kenako inagubuduzika. | Patsikuli dalayivala wagalimotoli, Aroni Simenti, amafuna kudutsa galimoto yomwe sikudziwika, koma analephera kuwongolera bwino galimotolo, kamba kothamangitsa kwambiri, kenako inagubuduzika. | female | |
Kutsatira izi, dalayivayo ndi anthu ena awiri, anavulala kwambiri m’mutu, ndipo anafera pamalo angoziyo. Pomwe anthu ena asanu ndi m’modzi (6), | Kutsatira izi, dalayivayo ndi anthu ena awiri, anavulala kwambiri m’mutu, ndipo anafera pamalo angoziyo. Pomwe anthu ena asanu ndi m’modzi (sikisi), | female | |
Omwe ndi Pria Mwale 32, Tamala Mithi 20, Sitayileni Mbewe 26, Atupele Mwenechanya 18, Yohane Mikayele 44 ndi Thandizo Muhango 23. | Omwe ndi Puriya Mwale sete-thu, Tamala Mithi tuwente, Sitayileni Mbewe tuwente-sikisi, Atupele Mwenechanya eyitini, Yohane Mikayele fote-folo ndi Thandizo Muhango tuwente-firi. | female | |
Anavulala kwambiri ndipo adatengedwera ku chipatala chachikulu cha Nkhotakota, kuti akalandire thandizo lamankhwala. | Anavulala kwambiri ndipo adatengedwera ku chipatala chachikulu cha Nkhotakota, kuti akalandire thandizo lamankhwala. | female | |
Nduna yazawulimi, Sam Kawale, yati ndiyokhutira ndi ulimi wachimanga chathirira womwe wakhala ukuchitika pamalo okwana ma hekitala 102 a company yopanga sugar ya Illovo ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota. | Nduna yazawulimi, Samu Kawale, yati ndiyokhutira ndi ulimi wachimanga chathirira womwe wakhala ukuchitika pamalo okwana ma hekitala wani handiredi and thu a kampani yopanga shuga ya Ilovo ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota. | female | |
Ndunayi yalankhula izi, itawona chimanaga chomwe chakololedwa pakadalipano ndipo chikusungidwa ku nkhokwe ya ADMARC ya Nkhunga m’bomali. | Ndunayi yalankhula izi, itawona chimanaga chomwe chakololedwa pakadalipano ndipo chikusungidwa ku nkhokwe ya ADIMAKI ya Nkhunga m’bomali. | female | |
Malingana ndi Kawale, izi zupherezera masomphenya adzikolino a Malawi 2063, olimbikitsa ulimi wathirira ndicholinga choti dzikolino lizikhala ndi chimanga chokwanira. | Malingana ndi Kawale, izi zupherezera masomphenya adzikolino a Malawi tuwente sikisite-firi, olimbikitsa ulimi wathirira ndicholinga choti dzikolino lizikhala ndi chimanga chokwanira. | female | |
Ndunayi yatinso, boma ndilodzipereka kuthandiza magulu alimi ndi mbalizina zokhudzidwa ngati akufuna kuyamba ulimi wa minda ikuluikulu. | Ndunayi yatinso, boma ndilodzipereka kuthandiza magulu alimi ndi mbalizina zokhudzidwa ngati akufuna kuyamba ulimi wa minda ikuluikulu. | female | |
Nduna yazaulimi Sam Kawale, yakwera ndenge ya company ya Illovo yomwe number yake ndi ZSLEC yomwe agwiritse ntchito poyendera malo a ulimi a kampaniyi. | Nduna yazaulimi Samu Kawale, yakwera ndenge ya kampani ya Ilovo yomwe nambala yake ndi ZEDI ESI ELO E SI yomwe agwiritse ntchito poyendera malo a ulimi a kampaniyi. | female | |
Motsogozedwa ndi mkulu wa company ya Illovo Jeremy Ngolombe, ndunayi ili limodzi ndi akuluakulua ena monga wachiwiri kwa Chancellor wa school ya ukachenjede ya LUANAR professor Kawunda. | Motsogozedwa ndi mkulu wa kampani ya Ilovo Jereme Ngolombe, ndunayi ili limodzi ndi akuluakulua ena monga wachiwiri kwa Tchansala wa sukulu ya ukachenjede ya LUWANA purofesa Kawunda. | female | |
Akamaliza kuyendera malowa, akukuakukuwa akhala akupita kukaona chimanga chomwe chikusungidwa ku nkhokwe ya ADMARC ya Nkhunga. | Akamaliza kuyendera malowa, akukuakukuwa akhala akupita kukaona chimanga chomwe chikusungidwa ku nkhokwe ya ADIMAKI ya Nkhunga. | female | |
M’phunzitsi wapasukulu ya ukachenjede ya LUANAR Dr, Thomas Nyanda, yemwe wakhala akutsogolera ntchito ya ulimi wathirira pamunda wachimanga ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota. | M’phunzitsi wapasukulu ya ukachenjede ya LUWANA Dokota, Thomasi Nyanda, yemwe wakhala akutsogolera ntchito ya ulimi wathirira pamunda wachimanga ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota. | female | |
Wati chimanga china chinayamba kukololedwa, pomwe china sichinafikepo. Dr. Nyanda watichimangachi, chinadzalidwa mosiyana. China chinadzalidwa pa 17 July, 2023, | Wati chimanga china chinayamba kukololedwa, pomwe china sichinafikepo. Dokota Nyanda watichimangachi, chinadzalidwa mosiyana. China chinadzalidwa pa sventini Julayi, tuwente-firi, | female | |
Pomwe china chinadzalidwa pa 24 August, 2023. Iye wati, chimanga chomwe chakololedwa pakadalipano chikusungidwa mu nkhokwe zaboma za bungwe logula ndi kugulitsa mbewu la ADMARC, ku Nkhunga m’bomali. | Pomwe china chinadzalidwa pa tuwente-folo Ogasiti, tuwente tuwente-firi. Iye wati, chimanga chomwe chakololedwa pakadalipano chikusungidwa mu nkhokwe zaboma za bungwe logula ndi kugulitsa mbewu la ADIMAKI ku Nkhunga m’bomali. | female | |
Malingana ndi chiyerekezo chake, pa hekitala iliyonse, pakuyembekezereka kukololedwachimanga chosachepera ma tone 7. | Malingana ndi chiyerekezo chake, pa hekitala iliyonse, pakuyembekezereka kukololedwachimanga chosachepera ma tone seveni. | female | |
Kamba ka mavuto achuma omwe akuta dziko la Malawi, asodzi m’boma la Nkhotakota, ati akukumana ndi mavuto ochuluka pamoyo wawo watsiku ndi tsiku zomwe ati zakolezeledwa ndi nthawi yotseka nyanja ya Malawi. | Kamba ka mavuto achuma omwe akuta dziko la Malawi, asodzi m’boma la Nkhotakota, ati akukumana ndi mavuto ochuluka pamoyo wawo watsiku ndi tsiku zomwe ati zakolezeledwa ndi nthawi yotseka nyanja ya Malawi. | female | |
Asodzi okhudzidwa ochokera m’madoko osiyanasiyana m’bomali, anakapereka chikalata cha madando, ku office ya bwanamkubwa ya khonsolo ya bomali. | Asodzi okhudzidwa ochokera m’madoko osiyanasiyana m’bomali, anakapereka chikalata cha madando, ku ofesi ya bwanamkubwa ya khonsolo ya bomali. | female | |
Ndikupempha kuti aganizire kusintha miyezi yotsekera nyanjayi, pofuna kuwathandiza kupeza zofunikira pamoyo wa tsiku ndi tsiku. | Ndikupempha kuti aganizire kusintha miyezi yotsekera nyanjayi, pofuna kuwathandiza kupeza zofunikira pamoyo wa tsiku ndi tsiku. | female | |
M’modzi mwa asodziwa Grecious Chirwa, Yemwe amachita usodzi wake padoko la Chipala m’bomali, wati kutseka nyanja kuchoka mwezi wa December kufika February, silikhala thandizo kwa iwo. | M’modzi mwa asodziwa Gireshiyasi Chirwa, yemwe amachita usodzi wake padoko la Chipala m’bomali, wati kutseka nyanja kuchoka mwezi wa Disembalar kufika Febuluwale, silikhala thandizo kwa iwo. | female | |
Kamba koti kuyambira mwezi wa March, kupita mtsogolo, kumakhala mphepo yamwera, zomwe zimatha kuchititsa kuti akhale miyezi yochuluka asakugwira ntchito. | Kamba koti kuyambira mwezi wa Machi, kupita mtsogolo, kumakhala mphepo yamwera, zomwe zimatha kuchititsa kuti akhale miyezi yochuluka asakugwira ntchito. | female | |
Iwo ati adindo akuyenera kulingalira zowunikira lamulo lotseka nyanjayi. Malingana ndi Chirwa, lamuloli lidapangidwa m’boma la Mangochi. | Iwo ati adindo akuyenera kulingalira zowunikira lamulo lotseka nyanjayi. Malingana ndi Chirwa, lamuloli lidapangidwa m’boma la Mangochi. | female | |
Komwe nyengo, kayendedwe ka mphepo komaso kukula kwa nyanja ndikosiyana ndi boma la Nkhotakota. Bwana mkubwa wakhonsolo yabomali Ben Matengeni Tono, wati madandowa apititsidwa kwa adindo oyenera. | Komwe nyengo, kayendedwe ka mphepo komaso kukula kwa nyanja ndikosiyana ndi boma la Nkhotakota. Bwana mkubwa wakhonsolo yabomali Beni Matengeni Tono, wati madandowa apititsidwa kwa adindo oyenera. | female | |
Bungwe lolimbikitsa chilungamo komanso mpikisano woyenerera pamalonda la Competition and Fair Trading Commission CFTC. | Bungwe lolimbikitsa chilungamo komanso mpikisano woyenerera pamalonda la kompitishonzi andi Fey Thireding'i komishoni (SI EFU TI SI). | female | |
Lati ndiKofunika kilimbikitsa kufalitsa uthenga okhudza mpikisano woyenera pamalonda ngati dziko likufuna kuthana ndi mchitidwe wophwanya malamulo pochita malonda. | Lati ndiKofunika kilimbikitsa kufalitsa uthenga okhudza mpikisano woyenera pamalonda ngati dziko likufuna kuthana ndi mchitidwe wophwanya malamulo pochita malonda. | female | |
Mneneri wabungweri, Innocent Herema, wati kusokonekera kwa chuma kamba ka ngozi zadzidzidzi monga namondwe wa Freddy, matenda a Cholera, komanso kutsika mphavu kwa ndalama yakwacha. | Mneneri wabungweri, Inosenti Herema, wati kusokonekera kwa chuma kamba ka ngozi zadzidzidzi monga namondwe wa Furedi, matenda a kolera, komanso kutsika mphavu kwa ndalama yakwacha. | female | |
Kwapangitsa kuti mchitidwe wochita malonda mosayenerera ukule. Mawu ake akudza pomwe dziko la Malawi likukumbukira nawo tsiku lolimbikitsa mpikisano woyenera pamalonda, omwe umachitika pa 5 December, chaka chilichonse. | Kwapangitsa kuti mchitidwe wochita malonda mosayenerera ukule. Mawu ake akudza pomwe dziko la Malawi likukumbukira nawo tsiku lolimbikitsa mpikisano woyenera pamalonda, omwe umachitika pa fayiai Disemba, chaka chilichonse. | female | |
Ndipo mwambo wa chakachino, ukukumbukiridwa pamutu woti ‘mpikisano woyenerapobwezeretsa chuma mchimake.’ Iye wati tsikuli likhazikitsa mwayi kuti adindo okhudzidwa abwere pamodzi. | Ndipo mwambo wa chakachino, ukukumbukiridwa pamutu woti ‘mpikisano woyenerapobwezeretsa chuma mchimake.’ Iye wati tsikuli likhazikitsa mwayi kuti adindo okhudzidwa abwere pamodzi. | female | |
Polimbana ndi mchitidwe wosatsatira malamulo pantchito zamalonda, ndi cholinga chofuna kuteteza ogula. Bwanamkubwa wa khonsolo ya mzinda wa Lilongwe, | Polimbana ndi mchitidwe wosatsatira malamulo pantchito zamalonda, ndi cholinga chofuna kuteteza ogula. Bwanamkubwa wa khonsolo ya mzinda wa Lilongwe, | female | |
Dr. Lawford Palani, wawuza gulu la anamwino, komanso aphunzitsi a primary, omwe sanalembedwe ntchito, kuti lisintha tsiku loyamba kuchita m’bindikiro omwe unakozedwa kuyamba pa 30 mwenzi uno. | Dokota. Lofodi Palani, wawuza gulu la anamwino, komanso aphunzitsi a purayimare, omwe sanalembedwe ntchito, kuti lisintha tsiku loyamba kuchita m’bindikiro omwe unakozedwa kuyamba pa sete mwenzi uno. | female | |
Kudzera mchikalata chomwe chatulutsidwa lolemba, Dr. Balani wati maunduna azawumoyo komanso maphunziro, akonza mkomano womwe uchitike pa 29, mwenzi uno. | Kudzera mchikalata chomwe chatulutsidwa lolemba, Dokota Palani wati maunduna azawumoyo komanso maphunziro, akonza mkomano womwe uchitike pa tuwente nayini, mwenzi uno. | female | |
Ofuna kumva zenizeni zomwe gululi likufunitsitsa boma litachita malingana ndi pempho lawo. Polankhulapo pa izi, mkhalapampando wagululi, Frank Kamwendo, | Ofuna kumva zenizeni zomwe gululi likufunitsitsa boma litachita malingana ndi pempho lawo. Polankhulapo pa izi, mkhalapampando wagululi, Furanki Kamwendo, | female | |
Wati ndizokhumudwitsa kamba koti mikomano ngati yomweyi, yakhala ikuchitika m’mbuyomu, koma simafikira zomwe gululi likufuna. | Wati ndizokhumudwitsa kamba koti mikomano ngati yomweyi, yakhala ikuchitika m’mbuyomu, koma simafikira zomwe gululi likufuna. | female | |
Komabe Kamwendo wati gululi litumiza nthumwi ku khonsolo ya mzindawu kuti akakambirane ngati pali kuthekera koti lipitilize ndi ganizo lochititsa m’bindikiro komanso kukakumana ndi adindo ochokera ku unduna wazaumoyo komanso maphunziro. | Komabe Kamwendo wati gululi litumiza nthumwi ku khonsolo ya mzindawu kuti akakambirane ngati pali kuthekera koti lipitilize ndi ganizo lochititsa m’bindikiro komanso kukakumana ndi adindo ochokera ku unduna wazaumoyo komanso maphunziro. | female | |
Mfumu Chitambo ya mdera la senior chief Mphonde, m’boma la Nkhotakota, yati ndiyodzipereka kuthetsa mawukwati a ana achichepere mderalake. | Mfumu Chitambo ya mdera la siniyo chifi Mphonde, m’boma la Nkhotakota, yati ndiyodzipereka kuthetsa mawukwati a ana achichepere mderalake. | female | |
Mfumuyi yalankhula izi pomwe akuluakulu ochokera kunthambi yophunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana ku unduna wamaboma ang’ono limodzi ndi chikhalidwe, | Mfumuyi yalankhula izi pomwe akuluakulu ochokera kunthambi yophunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana ku unduna wamaboma ang’ono limodzi ndi chikhalidwe, | female | |
Lero ali mderari kuyendera ntchito zomwe committee yophunzitsa anthu mdera la mfumu mphonde yakhala ikugwira. Committeeyi imagwiritsa ntchito zisudzo msukulu, | Lero ali mderari kuyendera ntchito zomwe komiti yophunzitsa anthu mdera la mfumu mphonde yakhala ikugwira. komitiyi imagwiritsa ntchito zisudzo msukulu, | female | |
Komanso misonkhano ya m’madera pofikira anthu ndi uthenga wokhudza kusintha kaganizidwe, kuphatikiza kulimbikitsa maphunziro pakati pa ana amderari. | Komanso misonkhano ya m’madera pofikira anthu ndi uthenga wokhudza kusintha kaganizidwe, kuphatikiza kulimbikitsa maphunziro pakati pa ana amderari. | female | |
Komitiyi yomwe yakhazikitsidwa m’mwezi wa February chakachino, cholingachake ndikulimbikitsa uthenga wokhudza kusintha kwa kaganizidwe pakati pa anthu, ngati mbali imodzi ya masomphenya adzikolino a Malawi 2063. | Komitiyi yomwe yakhazikitsidwa m’mwezi wa Feburuware chakachino, cholingachake ndikulimbikitsa uthenga wokhudza kusintha kwa kaganizidwe pakati pa anthu, ngati mbali imodzi ya masomphenya adzikolino a Malawi tuwente sikisite firi. | female | |
Bungwe lowona za mphavu yamagetsi ndi zambwezera ya Malawi Energy Regulatory Authority (MERA), layimitsa kaye ntchito zamalo omwetsera mafuta ya Mount Meru Chinsapo mu mzinda wa Lilongwe. | Bungwe lowona za mphavu yamagetsi ndi zambwezera ya Malawi Eneje Reguletare Oforite (MERA), layimitsa kaye ntchito zamalo omwetsera mafuta ya Mowunti Meru Chinsapo mu mzinda wa Lilongwe. | female | |
Kwamasiku makumi atatu 30, ati chifukwa chokakamiza anthu ogula mafuta, kuti azilipira ndalama ina yapamwamba. Chikalata chomwe bungwe la MERA latulutsa dzulo, | Kwamasiku makumi atatu sete, ati chifukwa chokakamiza anthu ogula mafuta, kuti azilipira ndalama ina yapamwamba. Chikalata chomwe bungwe la MERA latulutsa dzulo, | female | |
Bungweri linachita kafukufuku pamalo omwetsera mafutawa, ndipo lapeza kuti anthu ogula mafuta pamalowa, amakakamizidwa kupereka 5000 kwacha yowonjezera, | Bungweri linachita kafukufuku pamalo omwetsera mafutawa, ndipo lapeza kuti anthu ogula mafuta pamalowa, amakakamizidwa kupereka fayifi sauzandi kwacha yowonjezera, | female | |
ngati akufuna kugula mafuta wochuluka kuposa mulingo omwe malowa adayika kuti munthu adzugula. Pakadali ano bungweri lalimbikitsa anthu mdzikomuno. | ngati akufuna kugula mafuta wochuluka kuposa mulingo omwe malowa adayika kuti munthu adzugula. Pakadali ano bungweri lalimbikitsa anthu mdzikomuno. | female | |
Kuti azineneza ku bungweri akawona zinthu monga izi, zikuchitika pamalo aliwonse omwetsera mafuta mdzikomuno. Nduna yowona za chilungamo Titus Mvalo, | Kuti azineneza ku bungweri akawona zinthu monga izi, zikuchitika pamalo aliwonse omwetsera mafuta mdzikomuno. Nduna yowona za chilungamo Tayitasi Mvalo, | female | |
Yati undunawu wamaliza ntchito, yopanga ndondomeko zoyendetsera lamulo loyendetsera zipani la 2018, lomwe pachingerezi limatchedwa kuti political parties act. | Yati undunawu wamaliza ntchito, yopanga ndondomeko zoyendetsera lamulo loyendetsera zipani la tuwente eyitini, lomwe pachingerezi limatchedwa kuti politiko patezi akiti. | female | |
Mvalo wati, chatsala ndikupereka ndondomekozi ku committee yowona zamalamulo ya kunyumba yamalamulo, kuti iwunikirenso bwino. Mwazina lamuloli limathetsa anthu andale | Mvalo wati, chatsala ndikupereka ndondomekozi ku komiti yowona zamalamulo ya kunyumba yamalamulo, kuti iwunikirenso bwino. Mwazina lamuloli limathetsa anthu andale | female | |
Kupereka zinthu monga ndalama panthawi yamisonkhano yokopa anthu. Koma polankhulapo pankhaniyi, phungu wachigawo chapakati, m’boma la Thyolo Ben Phiri. | Kupereka zinthu monga ndalama panthawi yamisonkhano yokopa anthu. Koma polankhulapo pankhaniyi, phungu wachigawo chapakati, m’boma la Thyolo Beni Phiri. | female | |
Sakugwirizana ndiganizo loti ndondomekozi zidutse ku komitiyi, ponena kuti izi zichedwetsa kuti lamuloli liyambe kugwira ntchito. | Sakugwirizana ndiganizo loti ndondomekozi zidutse ku komitiyi, ponena kuti izi zichedwetsa kuti lamuloli liyambe kugwira ntchito. | female | |
Asodzi a boma la Nkhotakota, tsopano mabwato awo azikhala ndi chizindikiro cha utoto wa mtundu wakuda. Kutsatira ntchito yomwe nthambi yowona za usodzi mdzikomuno, yakhazikitsa. | Asodzi a boma la Nkhotakota, tsopano mabwato awo azikhala ndi chizindikiro cha utoto wa mtundu wakuda. Kutsatira ntchito yomwe nthambi yowona za usodzi mdzikomuno, yakhazikitsa. | female | |
Pa mkomano womwe nthambi ya wusodzi m’boma la Nkhotakota ndi bungwe la PACT Malawi pansi pa ntchito ya Refresh, anachititsa lachitatu, mkulu wa office yowona za usodzi m’bomali, Charles Mandala, | Pa mkomano womwe nthambi ya wusodzi m’boma la Nkhotakota ndi bungwe la PAKITI Malawi pansi pa ntchito ya Rifureshi, anachititsa lachitatu, mkulu wa ofesi yowona za usodzi m’bomali, Tchalosi Mandala, | female | |
Wati, ntchitoyi ndiyabwino kamba koti azithandizira kupereka chizindikiro cha mabwato a m’bomali. Woyendetsa ntchito za project ya refresh ku bungwe la pact Malawi m’boma la Nkhotakota. | Wati, ntchitoyi ndiyabwino kamba koti azithandizira kupereka chizindikiro cha mabwato a m’bomali. Woyendetsa ntchito za purojekiti ya rifureshi ku bungwe la pakiti Malawi m’boma la Nkhotakota. | female | |
Andrew Salapa, wapempha ansodzi kuti atsatire dongosolo latsopanoli, ponena kuti zikugwirizana ndi malamulo a usodzi mdzikomuno. | Anduru Salapa, wapempha ansodzi kuti atsatire dongosolo latsopanoli, ponena kuti zikugwirizana ndi malamulo a usodzi mdzikomuno. | female | |
Pa mkomano, panali adindo wochokera ku khonsolo ya boma la Nkhotakota, Makhansala, mafumu ndi adindo ena okhudzidwa mwa anthu ena. | Pa mkomano, panali adindo wochokera ku khonsolo ya boma la Nkhotakota, Makhansala, mafumu ndi adindo ena okhudzidwa mwa anthu ena. | female | |
Katswiri pankhani zaulimi, Tamani Nkhono Mvula, wachenjeza kuti dzikolino likumana ndi vuto lanjala chaka chamawa. | Katswiri pankhani zaulimi, Tamani Nkhono Mvula, wachenjeza kuti dzikolino likumana ndi vuto lanjala chaka chamawa. | female | |
Ngati boma siliyika ndondomeko zapadera zothandizira alimi, kutstira kukwera mtengo kwa zipangizo za ulimi. | Ngati boma siliyika ndondomeko zapadera zothandizira alimi, kutstira kukwera mtengo kwa zipangizo za ulimi. | female | |
Mawu a Mvula akudza pomwe zipangizo za ulimi monga feteleza ndi mbeu zina mdzikomuno, zakwera mtengo, zomwe zadza kamba kakutsika mphavu kwa ndalama yakwacha mdzikomuno. | Mawu a Mvula akudza pomwe zipangizo za ulimi monga feteleza ndi mbeu zina mdzikomuno, zakwera mtengo, zomwe zadza kamba kakutsika mphavu kwa ndalama yakwacha mdzikomuno. | female | |
Iye wati, kutsika kwa chiwerengero cha anthu omwe apindule nawo mundondomeko yogulitsa zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya AIP yachaka cha 2023-2024, kuchititsanso kuti alimi ochuluka | Iye wati, kutsika kwa chiwerengero cha anthu omwe apindule nawo mundondomeko yogulitsa zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya EAYIPI yachaka cha tuwente tuwente firi-tuwente tuwente folo, kuchititsanso kuti alimi ochuluka | female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.