audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Komanso a police kuti afufuze ndi kumanga omwe adachita mchitidwe wachipolowewu. Gulu la aphunzitsi a IPTE 13 ndi 14,
Komanso a polisi kuti afufuze ndi kumanga omwe adachita mchitidwe wachipolowewu. Gulu la aphunzitsi a IPITE Setini ndi fotini,
female
Omwe sadalembedwe ntchito m’boma la Nkhotakota, lawopseza kuti lichita m’bindikiro pa ma office akhonsolo ya bomali, pofuna kuwonetsa kusakondwa ndi ndondomeko yomwe khonsoloyi ikugwiritsa ntchito powalemba ntchito.
Omwe sadalembedwe ntchito m’boma la Nkhotakota, lawopseza kuti lichita m’bindikiro pa ma ofesi akhonsolo ya bomali, pofuna kuwonetsa kusakondwa ndi ndondomeko yomwe khonsoloyi ikugwiritsa ntchito powalemba ntchito.
female
Mneneri wa aphunzitsiwa Collings Chunga pomwe amapereka chikalata chamadando awo ku khonsoloyi m’mawa wa lero, wati ndowodabwa ndi ganizo la Khonsoloyi,
Mneneri wa aphunzitsiwa Koling'izi Chunga pomwe amapereka chikalata chamadando awo ku khonsoloyi m’mawa wa lero, wati ndowodabwa ndi ganizo la Khonsoloyi,
female
Polemba ntchito aphunzitsi asanu ndi anayi (9) okha a IPTE 13 ndi 14, m’malo molemba aphunzitsi 70, ngati momwe boma lidanenera.
Polemba ntchito aphunzitsi asanu ndi anayi (nayini) okha a IPITE setini ndi fotini, m’malo molemba aphunzitsi sevente, ngati momwe boma lidanenera.
female
Gululi likufunanso kudziwa ndondomeko yomwe khonsoloyi idagwiritsa ntchito, polemba ntchito aphunzitsiwa, maka polemba ntchito aphunzitsi ochuluka a IPTE 14 kusiya a IPTE 13.
Gululi likufunanso kudziwa ndondomeko yomwe khonsoloyi idagwiritsa ntchito, polemba ntchito aphunzitsiwa, maka polemba ntchito aphunzitsi ochuluka a IPITE fotini kusiya a IPITE setini.
female
Pomwe unduna wazamaphunziro udaneneratu kuti makhonsolo ayike pamtima, aphunzitsi a IPTE 13, omwe adali oyamba kutsiriza maphunziro awo.
Pomwe unduna wazamaphunziro udaneneratu kuti makhonsolo ayike pamtima, aphunzitsi a IPITE setini, omwe adali oyamba kutsiriza maphunziro awo.
female
Pakadalipano mneneri wa Khonsolo ya boma la Nkhotakota, Wongani Mkandawire, sadayankhulepo pankhaniyi. Bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Centre for Democracy and Economic Development Initiative CIDEDI,
Pakadalipano mneneri wa Khonsolo ya boma la Nkhotakota, Wongani Mkandawire, sadayankhulepo pankhaniyi. Bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Senta fo Demokirase andi Ikonomiki Divelopumenti Inishiyetivisi (SIDEDI),
female
Lapempha boma kudzera kwa mlangizi wake pa malamulo Thabo Chakaka Nyirenda, kuti liyambe layimitsa kaye dongosolo lopereka chipepeso kwa maanja awiri a anthu oganiziridwa kuti adawomberedwa ndi a police.
Lapempha boma kudzera kwa mlangizi wake pa malamulo Thabo Chakaka Nyirenda, kuti liyambe layimitsa kaye dongosolo lopereka chipepeso kwa maanja awiri a anthu oganiziridwa kuti adawomberedwa ndi a polisi.
female
Munkhalango ya Thuma m’boma la Salima. Mkulu wa bungwe la CIDEDI Sylvester Namiwa wanena izi pamsonkhano wa olemba nkhani mu mzinda wa Lilongwe,
Munkhalango ya Thuma m’boma la Salima. Mkulu wa bungwe la SIDEDI Silivesita Namiwa wanena izi pamsonkhano wa olemba nkhani mu mzinda wa Lilongwe,
female
Pomwe amalankhula kwa a Malawi pankhani zokhudza chitetezo cha mdziko. kutsatira imfa za anthu omwe akuphedwa mdzikomuno. Iye wati maanjawa, akuyenera kutetezedwa,
Pomwe amalankhula kwa a Malawi pankhani zokhudza chitetezo cha mdziko. kutsatira imfa za anthu omwe akuphedwa mdzikomuno. Iye wati maanjawa, akuyenera kutetezedwa,
female
monga momwe malamulo akunenera, pomwe dziko likudalira kuti mkafukufuku yemwe a police akuchita ufike kumapeto.
monga momwe malamulo akunenera, pomwe dziko likudalira kuti mkafukufuku yemwe a polisi akuchita ufike kumapeto.
female
Pakadalipano, Namiwa wapempha unduna wa chitetezo cha mdziko, kuti ukhazikitse kafukufuku wozama kufuna kupeza anthu omwe adachita izi, kamba koti a Malawi akukhala mwamantha.
Pakadalipano, Namiwa wapempha unduna wa chitetezo cha mdziko, kuti ukhazikitse kafukufuku wozama kufuna kupeza anthu omwe adachita izi, kamba koti a Malawi akukhala mwamantha.
female
Phungu wanyumba yamalamulo wa dera la kumpoto m’boma la Nkhotakota, Henley Chimunthu Banda, wadandawula ndi ma report oti chimanga chapititsidwa kumalo ogula ndi kugulitsidwa mbewu,
Phungu wanyumba yamalamulo wa dera la kumpoto m’boma la Nkhotakota, Henele Chimunthu Banda, wadandawula ndi malipoti oti chimanga chapititsidwa kumalo ogula ndi kugulitsidwa mbewu,
female
abungwe la ADMARK a Ngala mdera lake ponena kuti palibe malo omwe ali mdzinali m’bomali. Chimunthu Banda wati wapeza maripoti omwe akuwonetsa kuti matani achimanga pafupifupi 44, afika pamalowa.
abungwe la ADIMAKI a Ngala mdera lake ponena kuti palibe malo omwe ali mdzinali m’bomali. Chimunthu Banda wati wapeza maripoti omwe akuwonetsa kuti matani achimanga pafupifupi Ffote-folo, afika pamalowa.
female
Zomwe iye wati nzopereka mafunso ochuluka. Sipikala wakale wanyumba ya malamuloyu anadandawula pamkomano omwe unalipo pakati pa akomiti akunyumba yamalamulo,
Zomwe iye wati nzopereka mafunso ochuluka. Sipikala wakale wanyumba ya malamuloyu anadandawula pamkomano omwe unalipo pakati pa akomiti akunyumba yamalamulo,
female
Yomwe imawunika kagwiridwe ntchito ka makampani aboma ndi akuluakulu aku unduna wazaulimi, mnyumba yamalamulo mu mzinda wa Lilongwe.
Yomwe imawunika kagwiridwe ntchito ka makampani aboma ndi akuluakulu aku unduna wazaulimi, mnyumba yamalamulo mu mzinda wa Lilongwe.
female
Mkuyankha kwake, mkulu wa bungwe la ADMARK, Daniel Makata, wati vuto litha kukhala padzina la malowo, osati kuti chimangachi sichidafike mderari.
Mkuyankha kwake, mkulu wa bungwe la ADIMAKI, Daniyelo Makata, wati vuto litha kukhala padzina la malowo, osati kuti chimangachi sichidafike mderari.
female
Iye wati achita kafukufuku komanso kutsimikiza dzina lenileni la malowa lomwe limadziwika ndi anthu a mderaro. Nthambi ya ndende mdzikomuno,
Iye wati achita kafukufuku komanso kutsimikiza dzina lenileni la malowa lomwe limadziwika ndi anthu a mderaro. Nthambi ya ndende mdzikomuno,
female
Yati vuto lakusowa kwachakudya, lomwe linakhudza ndende ya Zomba latha, atakambirana ndi anthu omwe amaperekera chimanga pandendeyi. Mneneri wanthambi yandende mzikomuno Chimwemwe Shawah.
Yati vuto lakusowa kwachakudya, lomwe linakhudza ndende ya Zomba latha, atakambirana ndi anthu omwe amaperekera chimanga pandendeyi. Mneneri wanthambi yandende mzikomuno Chimwemwe Shawa,
female
Wati andendewa, akhala masiku awiri osadya, osati ngati momwe zimavekera kuti akhala masiku asanu (5).
Wati andendewa, akhala masiku awiri osadya, osati ngati momwe zimavekera kuti akhala masiku asanu (fayifi).
female
Shawah wati andendewa, amapatsidwa ndiwo zokha opanda nsima, pomwe nthambiyi imachilimika zothana ndi vutoli.
Shawah wati andendewa, amapatsidwa ndiwo zokha opanda nsima, pomwe nthambiyi imachilimika zothana ndi vutoli.
female
Magulu omenyera ufulu wa anthu, monga la Centre for Human Rights Education and Assistance CHREA, akhala akupempha boma kuti liwunikire ndikupeza njira zothetsera vutoli msanga.
Magulu omenyera ufulu wa anthu, monga la Senta fo Humani Rayitsi Ejukashoni andi Asisitansi (KHIRIYE), akhala akupempha boma kuti liwunikire ndikupeza njira zothetsera vutoli msanga.
female
Bwalo lamilandu la High Court, lolemba, labwezeretsa pa udindo mlembi wamkulu wachipani cha Democratic Progressive, Nicholas Dausi.
Bwalo lamilandu la Hayi khoti, lolemba, labwezeretsa pa udindo mlembi wamkulu wachipani cha Demokiratiki Purogiresivi, Nikolasi Dausi.
female
Oweruza mulandu Justice Mandala Mabulasa, muchikalata chomwe Umunthu FM yawona , wati chiletso chomwe chipani cha DPP chinayika chachotsedwa.
Oweruza mulandu Jasitisi Mandala Mabulasa, muchikalata chomwe Umunthu EFU EMU yawona , wati chiletso chomwe chipani cha DIPIPI chinayika chachotsedwa.
female
Ndipo Dausi yemwe ndi phungu wadera lachigawo chapakati m’boma la Mwanza, apitiriza kugwira ntchito yake ngati mlembi wamkulu wachipanichi.
Ndipo Dausi yemwe ndi phungu wadera lachigawo chapakati m’boma la Mwanza, apitiriza kugwira ntchito yake ngati mlembi wamkulu wachipanichi.
female
Komabe bwalo labwalori lati Dausi akuyenera kupereka chidziwitso muchipanichi msabata ziwiri zalamulo lomwe bwalori lapereka.
Komabe bwalo labwalori lati Dausi akuyenera kupereka chidziwitso muchipanichi msabata ziwiri zalamulo lomwe bwalori lapereka.
female
Kumayambiriro amwezi uno, chipani cha DPP chinalengeza kuti chachotsa mongoyembekezera Dausi yemwe ndi m’modzi mwa akuluakulu a committee yoyendetsa chipanichi.
Kumayambiriro amwezi uno, chipani cha DIPIPI chinalengeza kuti chachotsa mongoyembekezera Dausi yemwe ndi m’modzi mwa akuluakulu a komiti yoyendetsa chipanichi.
female
Ati kamba kochititsa zosemphana ndi malamulo oyendetsera chipanichi. Mlembi wa team ya Civil United Edgar Chipalanjira,
Ati kamba kochititsa zosemphana ndi malamulo oyendetsera chipanichi. Mlembi wa timu ya Sivo Yunayitedi Ediga Chipalanjira,
female
Wati timuyi yaganiza zosintha ndi kupatsa ntchito yina mphunzitsi wake Oscar Kaonda, kutsatira kusachita bwino kwa timuyi mu TNM super league.
Wati timuyi yaganiza zosintha ndi kupatsa ntchito yina mphunzitsi wake Osika Kawunda, kutsatira kusachita bwino kwa timuyi mu TI ENI EMU supa ligi.
female
Chipalanjira wati Civil ndi team yayikulu yomwe ikufunikira aphunzitsi amphavu, pomwe timuyi ikulimbana kuti isatuluke mu ligi.
Chipalanjira wati Sivo ndi timu yayikulu yomwe ikufunikira aphunzitsi amphavu, pomwe timuyi ikulimbana kuti isatuluke mu ligi.
female
Lolemba timu ya Civil, idalengeza kuti ipereka ntchito ina kwa Kaunda ndipo m’malomwake, yayikapo Alberce Makawa, yemwe azithandizidwa ndi Wilson Chidanti komanso Charles Ben.
Lolemba timu ya Sivo, idalengeza kuti ipereka ntchito ina kwa Kawunda ndipo m’malomwake, yayikapo Abasi Makawa, yemwe azithandizidwa ndi Wilisoni Chidanti komanso Tchalosi Beni.
female
Makawa yemwe amaphunzitsa timu ya Civil ya akazi, ayamba ntchito yake pomwe timuyi ili pa nambala 13 ndi ma points 25 pomwe yatsala ndi masewera asanu ndi atatu (8).
Makawa yemwe amaphunzitsa timu ya Sivo ya akazi, ayamba ntchito yake pomwe timuyi ili pa nambala setini ndi mapoyinti tuwente fayifi pomwe yatsala ndi masewera asanu ndi atatu (eyiti).
female
Bungwe lowona za mayeso la MANEB likukumbutsa makolo kuti akuyenera kulipira ndalama ya mayeso a sitandade 8, folomu 2 ndi 4 a chaka cha mawa
Bungwe lowona za mayeso la MANEBU likukumbutsa makolo kuti akuyenera kulipira ndalama ya mayeso a sitandade eiti, folomu thu ndi folo a chaka cha mawa
Female
kudzera munjira za makono zomwe bungweli linakhaziki tsa chaka chatha pofuna kupewa mchitidwe osakaza ndalamazi ndi adindo a sukulu zina
kudzera munjira za makono zomwe bungweli linakhaziki tsa chaka chatha pofuna kupewa mchitidwe osakaza ndalamazi ndi adindo a sukulu zina
Female
M’neneri wa bungwe la MANEB Mayamiko Chiwaya wauza Umunthu FM kuti izi zithandizila kuchepetsa nkhani zakudyedwa kwa ndalama komwe kunakhudza ophunzira mu chaka cha maphunziro changothachi
M’neneri wa bungwe la MANEBU Mayamiko Chiwaya wauza Umunthu Efuemu kuti izi zithandizila kuchepetsa nkhani zakudyedwa kwa ndalama komwe kunakhudza ophunzira mu chaka cha maphunziro changothachi
Female
Chiwaya wati makolo agwilitse ntchito njira ya Airtel Money, TNM Mpamba komanso njira zina zamakono zomwe ma banki amagwilitsila ntchito
Chiwaya wati makolo agwilitse ntchito njira ya eyatelo mane, Tieni emu Mpamba komanso njira zina zamakono zomwe ma banki amagwilitsila ntchito
Female
osati kupeleka kwa adindo a msukulu zomwe ana awo amaphunziro pofuna kupewa mchitidwe odyeledwa ndalamazi. Pakadali pano, mtsogoleri wa bungwe lomwe limayang’anila sukulu zoyima pazokha
osati kupeleka kwa adindo a msukulu zomwe ana awo amaphunziro pofuna kupewa mchitidwe odyeledwa ndalamazi. Pakadali pano, mtsogoleri wa bungwe lomwe limayang’anila sukulu zoyima pazokha
Female
Wycliff Chimwendo wati awonesetsa kuti sukulu zomwe zili pansi pa bungweli sizikhukhudzidwa ndi mtchitidwewu. Masana a lero, timu ya mpira wa miyendo ya akazi ya dziko lino
Wyayikilifi Chimwendo wati awonesetsa kuti sukulu zomwe zili pansi pa bungweli sizikhukhudzidwa ndi mtchitidwewu. Masana a lero, timu ya mpira wa miyendo ya akazi ya dziko lino
Female
yagonjetsa timu ya Seychelles ndi zigoli 17 kwa chilowere pamasewera opimana mphamvu omwe anachitikira pa bwalo la mpira ku Blantyre. Temwa Chawinga, Vanessa Chikupira ndi Chikondi Gondwe
yagonjetsa timu ya Seshelezi ndi zigoli seventini kwa chilowere pamasewera opimana mphamvu omwe anachitikira pa bwalo la mpira ku Bulantaya. Temwa Chawinga, Vanesa Chikupira ndi Chikondi Gondwe
Female
agoletsa zigoli zitatu aliyense, pomwe Sabina Thomu ndi Leticia Chinyamula agoletsa zigoli ziwiri aliyense
agoletsa zigoli zitatu aliyense, pomwe Sabina Thomu ndi Letisha Chinyamula agoletsa zigoli ziwiri aliyense
Female
Ireen Khumalo, Rose Kabzere, Sarah Mlimbika ndi Carol Mathyola nawo agoletsa chigoli chimodzi aliyese
Ailini Khumalo, Rosi Kabzere, Sara Mlimbika ndi Karo Mathyola nawo agoletsa chigoli chimodzi aliyese
Female
Matimuwa akuyembekezereka kukumananso Lachinayi sabata ino. Timu ya dziko linoyi ikusewera masewerowa pokonzekera mpikisano wa COSAFA
Matimuwa akuyembekezereka kukumananso Lachinayi sabata ino. Timu ya dziko linoyi ikusewera masewerowa pokonzekera mpikisano wa KOSAFA
Female
omwe ukuyembekezereka kuyamba pa 4 Okutobala chaka chino m’dziko la South Africa. Apolisi m’boma la Nkhotakota ati munthu yemwe thupi lake lapezeka atafa pafupi ndi sukulu ya sekondale
omwe ukuyembekezereka kuyamba pa folo Okutobala chaka chino m’dziko la Saufi afilika. Apolisi m’boma la Nkhotakota ati munthu yemwe thupi lake lapezeka atafa pafupi ndi sukulu ya sekondale
Female
ya Bishop Mtekateka m’bomali wadziwika kuti ndi Chikondi Chiphazi wa m’mudzi wa Phangwa m’dera la mfumu Malengachanzi m’bomali
ya Bishopu Mtekateka m’bomali wadziwika kuti ndi Chikondi Chiphazi wa m’mudzi wa Phangwa m’dera la mfumu Malengachanzi m’bomali
Female
M’neneri wa polisi ya Nkhotakota Paul Malimwe wati zotsatira za kuchipatara chachikulu cha Nkhotakota zawonetsa kuti malemuwa afa kaamba kotaya kwambiri magazi kutsatira kuvulala
M’neneri wa polisi ya Nkhotakota Po Malimwe wati zotsatira za kuchipatara chachikulu cha Nkhotakota zawonetsa kuti malemuwa afa kaamba kotaya kwambiri magazi kutsatira kuvulala
Female
Malingana ndi Malimwe, malemuwa anawombedwa ndi galimoto yomwe pakadali pano sikudziwika, ndipo apolisi anapeza thupili m’mawa wa Lolemba
Malingana ndi Malimwe, malemuwa anawombedwa ndi galimoto yomwe pakadali pano sikudziwika, ndipo apolisi anapeza thupili m’mawa wa Lolemba
Female
pomwe amagwira ntchito yawo yoyendera malo osiyanasiyana ngati mbali imodzi yopeleka chitetezo. Iye wati kafukufuku ofuna kupeza galimoto lomwe lakhudzidwa pa ngoziyi ndi dalaivala, ali mkati
pomwe amagwira ntchito yawo yoyendera malo osiyanasiyana ngati mbali imodzi yopeleka chitetezo. Iye wati kafukufuku ofuna kupeza galimoto lomwe lakhudzidwa pa ngoziyi ndi dalaivala, ali mkati
Female
Ogwira ntchito m'boma, kuyambira giledi C mpaka R, tsopano azipatsidwa alawansi yapadera yomwe boma lakhazikitsa
Ogwira ntchito m'boma, kuyambira giledi si mpaka ala, tsopano azipatsidwa alawansi yapadera yomwe boma lakhazikitsa
Female
Malingana ndi chikalata chomwe chasayinilidwa ndi mlembi ku nthambi yoremba anthu ntchito m'boma, Blessings Chilabade ndalamayi iziyambira K20, 000 mpaka K40, 000
Malingana ndi chikalata chomwe chasayinilidwa ndi mlembi ku nthambi yoremba anthu ntchito m'boma, Bulesing’izi Chilabade ndalamayi iziyambira Tuwente sauzande mpaka fote sauzande
Female
Chilabade wati omwe apindule ndi alawansiyi ayamba kulandira ndalamayi pa 1 Okutobala chaka chino. Iye wati achita izi pofuna kutukula miyoyo ya anthu ogwira ntchito m'boma
Chilabade wati omwe apindule ndi alawansiyi ayamba kulandira ndalamayi pa wani Okutobala chaka chino. Iye wati achita izi pofuna kutukula miyoyo ya anthu ogwira ntchito m'boma
Female
Gulu la anamwino omwe sanalembedwe ntchito m’dziko muno, labweleza kupempha boma kudzera kuunduna wazaumoyo kuti liwalembe ntchito
Gulu la anamwino omwe sanalembedwe ntchito m’dziko muno, labweleza kupempha boma kudzera kuunduna wazaumoyo kuti liwalembe ntchito
Female
Mlembi wa guluri Lusubiro Mwambene, wadandaura ndikuchepa kwa anamwino mzipatara za boma za m’dziko muno, pa nthawi yomwe pali chiwerengero chochuluka cha anamwino ndi azamba omwe akuvutika ndi ulova
Mlembi wa guluri Lusuwiro Mwambene, wadandaura ndikuchepa kwa anamwino mzipatara za boma za m’dziko muno, pa nthawi yomwe pali chiwerengero chochuluka cha anamwino ndi azamba omwe akuvutika ndi ulova
Female
Mwabene akuganiza kuti boma likutengerapo mwayi pakusowa kwa ntchito kwa anamwinowa pomawalemba ntchito mongoyembekezera nkumawapatsa ndalama zokwana k40, 000 pa mwezi, zomwe wati ndi nkhanza
Mwabene akuganiza kuti boma likutengerapo mwayi pakusowa kwa ntchito kwa anamwinowa pomawalemba ntchito mongoyembekezera nkumawapatsa ndalama zokwana fote sauzande kwacha pa mwezi, zomwe wati ndi nkhanza
Female
Guluri lapeleka kufika pa 5 mwezi wa Okutobala chaka chino kuti boma likhale litalemba ntchito anamwino okwana 5 thousand omwe akusowa ntchito
Guluri lapeleka kufika pa faifi mwezi wa Okutobala chaka chino kuti boma likhale litalemba ntchito anamwino okwana faifi sauzande omwe akusowa ntchito
Female
ndipo waopseza kuti anamwinowa adzayamba kunyanyala ntchito ngati pempho lawo siliyankhidwa. Pempho la anamwinowa lofuna kurembedwa ntchito
ndipo waopseza kuti anamwinowa adzayamba kunyanyala ntchito ngati pempho lawo siliyankhidwa. Pempho la anamwinowa lofuna kurembedwa ntchito
Female
likudza pomwe nawo a phunzitsi apulayimale a IPTE 13 ndi 14 apeleka pempho ngati lomweli ku unduna wazamaphunziro
likudza pomwe nawo a phunzitsi apulayimale a ipite fetini ndi fotini apeleka pempho ngati lomweli ku unduna wazamaphunziro
Female
Sukulu ya sekondale ya Lunzu mu mzinda wa Blantyre, yaletsedwa mongoyembekezera kuti isapelekenso chakudya chilichonse kwa ophunzira pasukuluyi
Sukulu ya sekondale ya Lunzu mu mzinda wa Bulantaya, yaletsedwa mongoyembekezera kuti isapelekenso chakudya chilichonse kwa ophunzira pasukuluyi
Female
ophunzira okwana 45 atadwala mwadzidzidzi m’mawa wa lero. M’neneri muunduna wa zamaphunziro Mphatso Nkuonera
ophunzira okwana fote faifi atadwala mwadzidzidzi m’mawa wa lero. M’neneri muunduna wa zamaphunziro Mphatso Nkuonera
Female
wati akuganizira kuti kudwala kwa ophunzirawa kwadza kaamba ka chakudya chomwe anapatsidwa. Iye wati mwa ophunzira 45-wa, omwe ambiri mwa iwo ndi atsikana
wati akuganizira kuti kudwala kwa ophunzirawa kwadza kaamba ka chakudya chomwe anapatsidwa. Iye wati mwa ophunzira fote faifi-wa, omwe ambiri mwa iwo ndi atsikana
Female
atatu okha ndi omwe agonekedwabe pa chipatara cha Mlambe Mission, koma ena onse atulutsidwa kaamba koti akupeza bwino ndipo abwelera kusukuluyi
atatu okha ndi omwe agonekedwabe pa chipatara cha Mlambe Mishoni, koma ena onse atulutsidwa kaamba koti akupeza bwino ndipo abwelera kusukuluyi
Female
M'mawa wa lero, munthu wina yemwe sakudziwika wapezeka atafa pa msewu opita ku nyanja ya Malawi pafupi ndi sukulu ya sekondale ya Bishop Mtekateka
M'mawa wa lero, munthu wina yemwe sakudziwika wapezeka atafa pa msewu opita ku nyanja ya Malawi pafupi ndi sukulu ya sekondale ya Bishopu Mtekateka
Female
m'mudzi mwa Phangwa m’dera la mfumu Malengachanzi m'boma la Nkhotakota. Anthu okhala moyandikana ndi malo omwe papezeka thupi la munthuyu, akuganizira kuti wachita kugundidwa ndi galimoto
m'mudzi mwa Phangwa m’dera la mfumu Malengachanzi m'boma la Nkhotakota. Anthu okhala moyandikana ndi malo omwe papezeka thupi la munthuyu, akuganizira kuti wachita kugundidwa ndi galimoto
Female
Koma m'neneri wa apolisi m'bomali Paul Malimwe wati ndizovuta kutsimikiza ngati munthuyo wagundidwadi ndi galimoto kapena ayi
Koma m'neneri wa apolisi m'bomali Po Malimwe wati ndizovuta kutsimikiza ngati munthuyo wagundidwadi ndi galimoto kapena ayi
Female
Iye wati zotsatira za kuchipatala ndizomwe zitsimikize chenicheni chomwe chadzetsa imfa ya munthuyu. Pakadali pano, thupi la munthuyu lili ku nyumba yachisoni pa chipatala chachikulu cha Nkhotakota

komwe likuyembekezereka kuyezedwa. Omwe akukonza mwambo wa chaka chino wa Ziyarah, ati zokonzekera zonse za mwambowu omwe uchitike sabata lamawa zili mchimake
komwe likuyembekezereka kuyezedwa. Omwe akukonza mwambo wa chaka chino wa Ziyara, ati zokonzekera zonse za mwambowu omwe uchitike sabata lamawa zili mchimake
Female
Mkhalapakati wa komiti ya Ziyarah Muhamad Shelfroma, wanena izi pa msonkhano wa olembankhani lero mu mzinda wa Blantyre
Mkhalapakati wa komiti ya Ziyara Muhamadi Shefuloma, wanena izi pa msonkhano wa olembankhani lero mu mzinda wa Bulantsya
Female
Shelfroma wati mwa zina, akhazikitsa ndondomeko zofuna kuthandiza anthu omwe akudwala pa chipatala cha Queen Elizabeth Central Hospital mu mzinda wa Blantyre
Shefuloma wati mwa zina, akhazikitsa ndondomeko zofuna kuthandiza anthu omwe akudwala pa chipatala cha kwini elizabefi sentilo hosipito mu mzinda wa Bulantaya
Female
ngati njira imodzi yokodwerera tsiku lomwe mtumiki Muhamad anabadwa. Iye wati chikondwelero cha chaka chino chikhala chosiyana ndi cha chaka chatha
ngati njira imodzi yokodwerera tsiku lomwe mtumiki Muhamadi anabadwa. Iye wati chikondwelero cha chaka chino chikhala chosiyana ndi cha chaka chatha
Female
pomwe wati chaka chatha, mwambowu unakhudzidwa ndi nthenda ya Covid-19 zomwe zinakhudza anthu ochuluka kuti asakhale nawo pa mdipiti wa Ziyarah
pomwe wati chaka chatha, mwambowu unakhudzidwa ndi nthenda ya Kovidi-naintini zomwe zinakhudza anthu ochuluka kuti asakhale nawo pa mdipiti wa Ziyara
Female
Bungwe lomwe limalimbana ndi mchitidwe ogwiritsa ntchito mankhwala ozunguza ubongo la Drug Fight Malawi lati kusowekera kwa ndalama ndi vuto lomwe likukhudza malingaliro a bungweri
Bungwe lomwe limalimbana ndi mchitidwe ogwiritsa ntchito mankhwala ozunguza ubongo la Dilagi faiti Malawi lati kusowekera kwa ndalama ndi vuto lomwe likukhudza malingaliro a bungweri
Female
ofuna kufikira achinyamata omwe akuphunzira msukulu za sekondale ndi uthenga okhudza kuipa kogwiritsa ntchito mankhwala ozonguza bongo
ofuna kufikira achinyamata omwe akuphunzira msukulu za sekondale ndi uthenga okhudza kuipa kogwiritsa ntchito mankhwala ozonguza bongo
Female
Nelson Zakeyu, mkulu wa bungweri, wati kafukufuku yemwe bungweri linachita posachedwapa msukulu zina za sekondale za boma
Neosoni Zakeyu, mkulu wa bungweri, wati kafukufuku yemwe bungweri linachita posachedwapa msukulu zina za sekondale za boma
Female
wawonetsa kuti pafupifupi ophunzira 60 pa 100 aliwonse amagwiritsa ntchito mankhwala ozunguza ubongo monga mowa komanso fodya
wawonetsa kuti pafupifupi ophunzira sikisite pa wani handiledi aliwonse amagwiritsa ntchito mankhwala ozunguza ubongo monga mowa komanso fodya
Female
Zakeyu wati mchitidwewu ndi odandaulitsa, ndipo iye anadandaula ndi kusowekera kwa chidwi pakati pa adindo osiyanasiyana pofuna kuthana ndi mchitidweu
Zakeyu wati mchitidwewu ndi odandaulitsa, ndipo iye anadandaula ndi kusowekera kwa chidwi pakati pa adindo osiyanasiyana pofuna kuthana ndi mchitidweu
Female
Apa, iye wapempha mabungwe komanso anthu omwe ali ndikuthekera kuti agwilire ntchito limodzi komanso achinyamata eni ake kuti apewe mchitidwewu
Apa, iye wapempha mabungwe komanso anthu omwe ali ndikuthekera kuti agwilire ntchito limodzi komanso achinyamata eni ake kuti apewe mchitidwewu
Female
Oyankhulapo pa nkhani za masewero m’dziko muno apempha kuti pakhazikitsidwe ndondomeko za nthawi yaitali zakagwiridwe ka ntchito zopititsa patsogolo masewero a mpira wa miyendo komaso manja

M’modzi mwa anthuwa Anthony Msukwa wayalankhula izi kutsatira momwe matimu a dziko lino akhalira pa mndandanda wa maiko pa nkhani za masewero
M’modzi mwa anthuwa Antone Msukwa wayalankhula izi kutsatira momwe matimu a dziko lino akhalira pa mndandanda wa maiko pa nkhani za masewero
Female
pomwe timu ya mpira wa miyendo komanso manja akakamilabe pa nambala 123 komanso 6 pa dziko lonse
pomwe timu ya mpira wa miyendo komanso manja akakamilabe pa nambala wani handiledi andi twente fili komanso sikisi pa dziko lonse
Female
Msukwa wati masewero m’dziko muno akhala asakuchita bwino kaamba kogwiritsa ntchito ndondomeko za kanthawi kochepa
Msukwa wati masewero m’dziko muno akhala asakuchita bwino kaamba kogwiritsa ntchito ndondomeko za kanthawi kochepa
Female
zomwe zimadza kaamba ka nthawi yochepa yomwe atsogoleri osankhidwa omwe amayendetsa masewero amakhala
zomwe zimadza kaamba ka nthawi yochepa yomwe atsogoleri osankhidwa omwe amayendetsa masewero amakhala
Female
Iye wati dziko lino lili ndi atsogoleri a masewero a masomphenya koma kusowa kwa ndondomeko za nthawi yaitali sikungathandize matimu a Flames komaso Queens kupita patali
Iye wati dziko lino lili ndi atsogoleri a masewero a masomphenya koma kusowa kwa ndondomeko za nthawi yaitali sikungathandize matimu a Fulemuzi komaso Kwinzi kupita patali
Female
Chipatara chachikulu cha m’boma la Zomba chati ophunzira wa pa sukulu ya ukachenjede ya University Malawi (UNIMA) wapezeka ndi nthenda ya Kolera
Chipatara chachikulu cha m’boma la Zomba chati ophunzira wa pa sukulu ya ukachenjede ya Yunivesite ofu Malawi (YUNIMA) wapezeka ndi nthenda ya Kolera
Female
Arnold Mndalira, m’neneri wachipatarachi, wauza Umunthu FM kuti m’modzi mwa ophunzirayu amaonetsa zizindikiro za nthenda ya Kolera
Anodi Mndalira, m’neneri wachipatarachi, wauza Umunthu Efuemu kuti m’modzi mwa ophunzirayu amaonetsa zizindikiro za nthenda ya Kolera
Female
ndipo anayezedwa Lachinayi pomwe zotsatira zake zawonetsa kuti ndi Kolera. Mndalira wati ophunzirayu ndi wa m’dera la Chikanda m’boma la Zomba
ndipo anayezedwa Lachinayi pomwe zotsatira zake zawonetsa kuti ndi Kolera. Mndalira wati ophunzirayu ndi wa m’dera la Chikanda m’boma la Zomba
Female
Iye wati akuluakulu azaumoyo akhazikitsa ntchito yophunzitsa anthu za kapewedwe ka nthendayi kuti isafalikire m’madera ena m’derali
Iye wati akuluakulu azaumoyo akhazikitsa ntchito yophunzitsa anthu za kapewedwe ka nthendayi kuti isafalikire m’madera ena m’derali
Female
Lachinayi sabata lino, boma la Karonga lalembetsanso munthu m’modzi odwala nthenda ya Kolera atayezedwa pa 19 mwezi uno
Lachinayi sabata lino, boma la Karonga lalembetsanso munthu m’modzi odwala nthenda ya Kolera atayezedwa pa naintini mwezi uno
Female
Ku Dowa, ophunzira apasukulu yomwe siyaboma ya Robert Brake atentha midada ina yophunziliramo pa sukuluyi usiku wathawu
Ku Dowa, ophunzira apasukulu yomwe siyaboma ya Lobati Buleki atentha midada ina yophunziliramo pa sukuluyi usiku wathawu
Female
Ophunzira ena pa sukuluyi awuza Umunthu FM kuti izi zachitika pomwe sakukondwera ndi ena mwa malamulo omwe sukuluyi yakhazikitsa
Ophunzira ena pa sukuluyi awuza Umunthu Efuemu kuti izi zachitika pomwe sakukondwera ndi ena mwa malamulo omwe sukuluyi yakhazikitsa
Female
Izi zikuchitika pomwe sukuluyi yasintha mphunzitsi wa mkulu posachedwapa. M'neneri wa polisi ya Dowa, Alice Sitima wati afotokoza zambiri apolisi akachita kafukufuku wa zomwe zachitika
izi zikuchitika pomwe sukuluyi yasintha mphunzitsi wa mkulu posachedwapa. M'neneri wa polisi ya Dowa, Alisi Sitima wati afotokoza zambiri apolisi akachita kafukufuku wa zomwe zachitika
Female
Yemwe amayankhulapo pankhani zakaganizidwe kangwiro Dr. Chiwoza Bandawe wati mpofunika kuti boma liganizire zolemba anamwino ndi madotolo ochuluka
Yemwe amayankhulapo pankhani zakaganizidwe kangwiro Dokota Chiwoza Bandawe wati mpofunika kuti boma liganizire zolemba anamwino ndi madotolo ochuluka
Female
owona zamatenda okhudza kaganizidwe kangwiro, ngati njira imodzi yothanirana ndi vutoli m’dziko muno. Mawu a Dr Bandawe, akudza pomwe dziko lino likukumbukira nawo tsiku la nthenda ya mu ubongo
owona zamatenda okhudza kaganizidwe kangwiro, ngati njira imodzi yothanirana ndi vutoli m’dziko muno. Mawu a Dokota Bandawe, akudza pomwe dziko lino likukumbukira nawo tsiku la nthenda ya mu ubongo
Female
yomwe imakhudza kaganizidwe kangwiro yotchedwa “Alzheimer” m’chingerezi, pa mutu oti Sikufulumira Sikuchedwa omwe cholinga chake ndikulimbikitsa kupewa komanso kuchiza vutoli mwansanga
yomwe imakhudza kaganizidwe kangwiro yotchedwa Azemiya m’chingerezi, pa mutu oti Sikufulumira Sikuchedwa omwe cholinga chake ndikulimbikitsa kupewa komanso kuchiza vutoli mwansanga
Female
Malingana ndi Dr Bandawe, kuchuluka kwa chiwerengero cha matenda okhudza kaganizidwe kangwiro ndi kaamba kakuchepa kwa akadaulo omwe amathandizira kuchiza matendawa
Malingana ndi Dokota Bandawe, kuchuluka kwa chiwerengero cha matenda okhudza kaganizidwe kangwiro ndi kaamba kakuchepa kwa akadaulo omwe amathandizira kuchiza matendawa
Female
ndipo wati ichi nchifukwa chake akufuna kuti boma liganizire zolemba chiwerengero chochuluka cha akadaulowa. Pogwilizana ndi Dr Bandawe, oyankhulapo pa nkhani zaumoyo Maziko Matemba
ndipo wati ichi nchifukwa chake akufuna kuti boma liganizire zolemba chiwerengero chochuluka cha akadaulowa. Pogwilizana ndi Dokota Bandawe, oyankhulapo pa nkhani zaumoyo Maziko Matemba
Female
akuganiza kuti mpofunika kuti dziko lino lichilimike pa nkhani yofalitsa mauthenga osiyanasiyana okhudza matenda omwe amakhudza kaganizidwe kangwiro, omwe akukhudza anthu ochuluka m’dziko muno
akuganiza kuti mpofunika kuti dziko lino lichilimike pa nkhani yofalitsa mauthenga osiyanasiyana okhudza matenda omwe amakhudza kaganizidwe kangwiro, omwe akukhudza anthu ochuluka m’dziko muno
Female
Unduna owona zokopa alendo wati ukugwira ntchito ndi unduna owona zachilungamo, maka pofuna kusintha lamulo lokhudza nyama zotetezedwa
Unduna owona zokopa alendo wati ukugwira ntchito ndi unduna owona zachilungamo, maka pofuna kusintha lamulo lokhudza nyama zotetezedwa
Female
pomwe akufuna kuti nkhani yokhudza chipepeso kwa anthu omwe avulazidwa kapena kuphedwa ndi nyamazi ikhale m’malamulo. Nduna muundunawu Vera Kamtukule yayankhura izi Lachitatu m’boma la Kasungu
pomwe akufuna kuti nkhani yokhudza chipepeso kwa anthu omwe avulazidwa kapena kuphedwa ndi nyamazi ikhale m’malamulo. Nduna muundunawu Vera Kamtukule yayankhura izi Lachitatu m’boma la Kasungu
Female
komwe inakapepesa maanja a anthu omwe anakhudzidwa pa mikangano yomwe yakhala ikuchitika pakati pa anthu ndi nyama m’bomali. Mwa zina, Kamtukule wati pofuna kuthana ndi mikanganoyi
komwe inakapepesa maanja a anthu omwe anakhudzidwa pa mikangano yomwe yakhala ikuchitika pakati pa anthu ndi nyama m’bomali. Mwa zina, Kamtukule wati pofuna kuthana ndi mikanganoyi
Female
boma mogwilizana ndi nthambi zokhuzidwa pa nkhani ya nyama zakutchile likumanga mpanda wa nyesi yamagetsi kuti nyamazi zisamatuluke munkhalangoyi
boma mogwilizana ndi nthambi zokhuzidwa pa nkhani ya nyama zakutchile likumanga mpanda wa nyesi yamagetsi kuti nyamazi zisamatuluke munkhalangoyi
Female