audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
izi amayankhula pamene pali kusamvana kwa masapota a mchigawo cha pakati maka pameneso inachoka ndi ma points awiri pamene imakasewera ma game awiri ndi Mafco komaso Civil
izi amayankhula pamene pali kusamvana kwa masapota a mchigawo cha pakati maka pameneso inachoka ndi ma pointsi awiri pamene imakasewera ma gemu awiri ndi Mafuko komaso sivo
Female
Poyankhulapo a Chitedze ati aliyese akudziwa bwino ntchito zawo kuti manja awo samatuluka chabe koma chofunika ndikupatsidwa mpata kuti agwire ntchito yawo momasuka
Poyankhulapo a Chitedze ati aliyese akudziwa bwino ntchito zawo kuti manja awo samatuluka chabe koma chofunika ndikupatsidwa mpata kuti agwire ntchito yawo momasuka
Female
Iye walonjeza kuti akapatsidwa mpata anthu awona zotsatira zabwino ndipo alimbikitsa ma zone kugwira ntchito yawo bwino. Iye anapitiliza kunena kuti board yawo ikhale ndi mgwilizano wabwino kuti mphamvu zigawidwe moyenera
Iye walonjeza kuti akapatsidwa mpata anthu awona zotsatira zabwino ndipo alimbikitsa ma zoni kugwira ntchito yawo bwino. Iye anapitiliza kunena kuti bodi yawo ikhale ndi mgwilizano wabwino kuti mphamvu zigawidwe moyenera
Female
Rodrick Chitedze anadziwika mu 2017 pamene team ya Nyerere inatenga TNM super league kuchokera mu thawi imeneyo team yankhala ikuvutika kuti ipeze mwayi wa chinkho chilichonse
Lodiliki Chitedze anadziwika mu twente seventini pamene timu ya Nyerere inatenga Tieniemu supa ligi kuchokera mu thawi imeneyo timu yankhala ikuvutika kuti ipeze mwayi wa chinkho chilichonse
Female
Pamene dziko lino likukozekera kulandira alendo ozachita masewera anyamata a achisodzera mu December, Amene akuyendesa zokonzera mwambowu a African Union Sports Council
Pamene dziko lino likukozekera kulandira alendo ozachita masewera anyamata a achisodzera mu Disemba, Amene akuyendesa zokonzera mwambowu a afulikani yuniyoni sipotsi khanso
Female
apereka malire mwezi wa October kuti dziko lino likhale kuti lamalizitsa ntchito yokoza mwabwalo onse ochititsira masewerowa
apereka malire mwezi wa okutoba kuti dziko lino likhale kuti lamalizitsa ntchito yokoza mwabwalo onse ochititsira masewerowa
Female
Mabwalow omwe akuyembekezeka kudzachititsa masewerowa ndi monga Silver, Greeven Sayenda indoor complex komanso Kamuzu Institute komwe kukhale masewero osambira
Mabwalowa omwe akuyembekezeka kudzachititsa masewerowa ndi monga Siliva, Gilivini Sayenda inido kompulekisi komanso Kamuzu Insichuti komwe kukhale masewero osambira
Female
Wapampando wa gulu loyendetsa ntchito yamasewera wosewa kapena kuti Region 5 a Dennis Mondela anati akuona kuti ntchito yokozekerayi ikuyenda bwino ndipo chilichonse chili mchimake
Wapampando wa gulu loyendetsa ntchito yamasewera wosewa kapena kuti lijoni faifi a Denisi Mondela anati akuona kuti ntchito yokozekerayi ikuyenda bwino ndipo chilichonse chili mchimake
Female
ndipo akukhulupilira kuti zithu zikhala zapamwamba kwambiri. Poyankhulapo nduna ya za achinyamata ndi masewera a Richard Chimwendo Banda , ponkhazikitsa mpikisanowu
ndipo akukhulupilira kuti zithu zikhala zapamwamba kwambiri. Poyankhulapo nduna ya za achinyamata ndi masewera a litchadi Chimwendo Banda , ponkhazikitsa mpikisanowu
Female
anati uwu ndi mwayi ku dziko la Malawi chifukwa udzapindula kwambiri muzochitika zosiyanasiyana, monga kukhala ndi mabwalo abwino, malo ogona abwino komanso ndalama zakunja
anati uwu ndi mwayi ku dziko la Malawi chifukwa udzapindula kwambiri muzochitika zosiyanasiyana, monga kukhala ndi mabwalo abwino, malo ogona abwino komanso ndalama zakunja
Female
koma a Chimwendo apempha kuti a Malawi tikhale wogwilizana. Maiko omwe akudzatenga nawo mbali mu region 5 youth games ndi Lesotho, Angola, Botswana, Eswatini, Mozambique, Namibia, South Africa, Zambia, Zimbabwe ndi Malawi
koma a Chimwendo apempha kuti a Malawi tikhale wogwilizana. Maiko omwe akudzatenga nawo mbali mu lijoni faifi yufi gemuzi ndi Lesotho, Angola, Botswana, Eswatini, Mozambiki, Namibia, saufi afilika, Zambia, Zimbabwe ndi Malawi
Female
Masewera omwe akuyembekezeka kudzakhalapo ndi monga; Basket ball, Volleyball, Netball, Football, Taekwando, Judo ndi Tennis. Ndipo masewerawa akuyembekezeka kuzachitika mwezi wa December kuno kwathu ku Malawi
Masewera omwe akuyembekezeka kudzakhalapo ndi monga; Basiketobo, volebo, netibo, futubo, taikwando, Judo ndi Tenisi. Ndipo masewerawa akuyembekezeka kuzachitika mwezi wa Deisemba kuno kwathu ku Malawi
Female
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani Cha UTM, Dr. Saulos Chilima wati ndi okhumudwa ndi zina zomwe ena mwa anthu achipani Cha Malawi Congress Party (MCP) akupanga
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani Cha Yutiemu, Dokota Saulosi Chilima wati ndi okhumudwa ndi zina zomwe ena mwa anthu achipani Cha Malawi kongelesi pate (emusipi) akupanga
Female
zomwe ndi zosemphana ndi mgwirizano wawo wa Tonse alliance.A Chilima ati iwo ndi Dr. Lazarus Chakwera unamvana kuti a Chakwera adzalamulira zaka zisanu
zomwe ndi zosemphana ndi mgwirizano wawo wa Tonse alayansi. A Chilima ati iwo ndi Dokota Lazalasi Chakwera unamvana kuti a Chakwera adzalamulira zaka zisanu
Female
kenako adzapereka mpata kwa a Chilima kuti nawo alamulirenso zaka zina zisanu pansi pa mgwirizano wawo wa Tonse alliance
kenako adzapereka mpata kwa a Chilima kuti nawo alamulirenso zaka zina zisanu pansi pa mgwirizano wawo wa Tonse alayansi
Female
Kuonjezera apo Mtsogoleri wa UTM yu watinso nkofunika kuti malamulo aunikiridwenso kuti ngakhale mtsogoleri wa dziko adzitha kuyankha milandu adakali pampando
Kuonjezera apo Mtsogoleri wa yutiemu yu watinso nkofunika kuti malamulo aunikiridwenso kuti ngakhale mtsogoleri wa dziko adzitha kuyankha milandu adakali pampando
Female
osadikira kuti adzachoke paudindowu ndipo asamakhale ndi mphanvu ngati Pali mulandu okuti ayankhepo. Ngati anzathuwa akufuna kuti mgwilizanowu uthe nzotheka angothetsa tikatere tikavotenso
osadikira kuti adzachoke paudindowu ndipo asamakhale ndi mphanvu ngati Pali mulandu okuti ayankhepo. Ngati anzathuwa akufuna kuti mgwilizanowu uthe nzotheka angothetsa tikatere tikavotenso
Female
Watero wachiwiri kwa Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Saulos Chilima pamene amayankhapo mu mzinda wa Lilongwe pa mphekesera yomwe ikunveka kuti akukhudzidwa ndi za katangale
Watero wachiwiri kwa Mtsogoleri wa dziko lino Dokota Saulosi Chilima pamene amayankhapo mu mzinda wa Lilongwe pa mphekesera yomwe ikunveka kuti akukhudzidwa ndi za katangale
Female
Dr Chakwera ati kumbali yawo ndiodzidzimuka kwambiri kuti anthu ena omwe akugwira nawo ntchito akutchulidwa ku mabwalo amilandu akunja powaganizira kuti adachita za katangale
Dokota Chakwera ati kumbali yawo ndiodzidzimuka kwambiri kuti anthu ena omwe akugwira nawo ntchito akutchulidwa ku mabwalo amilandu akunja powaganizira kuti adachita za katangale
Female
Mtsogoleri'yu akuyankhula izi potsatira kutchulidwa kwa akuluakulu angapo a boma omwe akuganizilidwa kuti adapanga za katangale ndi Zunneth Sattar
Mtsogoleri'yu akuyankhula izi potsatira kutchulidwa kwa akuluakulu angapo a boma omwe akuganizilidwa kuti adapanga za katangale ndi Zunefi Sata
Female
Akuluakulu'wa ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Saulos Chilima, Mkulu wa Malawi police service George Kainja, mkulu oyang'anira ogwira ntchito ku nyumba zaboma Chris Chaima Banda komanso ena ambiri
Akuluakulu'wa ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Saulosi Chilima, Mkulu wa Malawi polisi sevisi Joji Kainja, mkulu oyang'anira ogwira ntchito ku nyumba zaboma khilisi Chaima Banda komanso ena ambiri
Female
Dr Chakwera alengeza ndondomeko izi pofuna kuthandiza pa ntchito yosamala chuma cha boma. Maulendo achisawawa akuluakulu a boma achepetsedwa kufika pa maulendo atatu chaka chino. Osagawa ma allowance mwachisawawa
Dokota Chakwera alengeza ndondomeko izi pofuna kuthandiza pa ntchito yosamala chuma cha boma. Maulendo achisawawa akuluakulu a boma achepetsedwa kufika pa maulendo atatu chaka chino. Osagawa ma alawansi mwachisawawa
Female
Popita kunja, akuluakulu a boma adzikwera ndege Ku malo ofanana ndi anthu wamba. Ma board aboma asakumane kodutsa kanayi chaka chino. Mafuta a galimoto opita kwa nduna atsitsidwa ndi 20 percent
Popita kunja, akuluakulu a boma adzikwera ndege Ku malo ofanana ndi anthu wamba. Ma board aboma asakumane kodutsa kanayi chaka chino. Mafuta a galimoto opita kwa nduna atsitsidwa ndi twente pelesenti
Female
Mafuta aboma a galimoto adzituluka pokhapo pomwe akufunika. Galimoto zaboma zisayende pa nsewu kuyambira 6 koloko madzulo
Mafuta aboma a galimoto adzituluka pokhapo pomwe akufunika. Galimoto zaboma zisayende pa nsewu kuyambira sikisi koloko madzulo
Female
Nthambi zaboma siziloledwa kugula galimoto zatsopano. Boma silipeleka ntchito zatsopano Ku kampani. Osagula katundu wa wamba kunja. Ndi zina zambiri
Nthambi zaboma siziloledwa kugula galimoto zatsopano. Boma silipeleka ntchito zatsopano Ku kampani. Osagula katundu wa wamba kunja. Ndi zina zambiri
Female
Bungwe la National Registration Bureau Labweza 800 Million kwa Treasury. NRB likuti labwenza ndalama zokwanila 800 million
Bungwe la nesholo lejisitileshoni byulo Labweza eiti handede miliyoni kwa Thilezyale. Enialabi likuti labwenza ndalama zokwanila eiti handede miliyoni
Female
imene idalandilidwa kuchoka ku ma akaunti a Treasury mu 2020, A Director a NRB Mphatso Sambo atsimikimiza za Uthengawu
imene idalandilidwa kuchoka ku ma akaunti a thilezyale mu twente twente, A dailekita a enialabi Mphatso Sambo atsimikimiza za Uthengawu
Female
Iwo anena kuti, izi zidachitika mu April Chaka Cha 2020 pamene NRB idauza Boma likufuna ndalama zowonjezera zokwanila 800 million
Iwo anena kuti, izi zidachitika mu epulo Chaka Cha twente twente pamene enialabi idauza Boma likufuna ndalama zowonjezera zokwanila eiti handede miliyoni
Female
pa ntchito zomwe adakonza ndipo NRB idalandila ndalama zokwana Mk1.6 Biliyion imene idali yopyola mulingo idafuna iyo
pa ntchito zomwe adakonza ndipo enialabi idalandila ndalama zokwana wani pointi sikisi miliyoni kwacha imene idali yopyola mulingo idafuna iyo
Female
Izi zaululika pamene bungwe la Public Appointments Committee (PAC) lidayitanisa akulu akulu aku National Registration Bureau (NRB) kuti akafotokoze zandondomekoyi
Izi zaululika pamene bungwe la Pabuliki apointimetsi komiti (PAKI) lidayitanisa akulu akulu aku Neshono lejisitileshoni Byulo (enialabi) kuti akafotokoze zandondomekoyi
Female
zayambika, mitengo ya sugar yakwera. Kampani yopanga sugar ya Illovo sugar Malawi yalengeza kuti mitengo ya sugar yakwera kuyambira lero
zayambika, mitengo ya shuga yakwera. Kampani yopanga shuga ya Ilovo shuga Malawi yalengeza kuti mitengo ya shuga yakwera kuyambira lero
Female
Chikalata chomwe kampaniyi yatulutsa chati anthu akonzeke kugula sugar wa Brown okwana 1 KG pa mtengo osachepera 1,100 kwacha
Chikalata chomwe kampaniyi yatulutsa chati anthu akonzeke kugula shuga wa Bulauni okwana wani keiji pa mtengo osachepera wani sauzande wanihandiledi kwacha
Female
Izi zadza patangotha masiku ochepa ndalama ya dziko lino ya kwacha itachepetsedwa mphamvu ndi 25 percent
Izi zadza patangotha masiku ochepa ndalama ya dziko lino ya kwacha itachepetsedwa mphamvu ndi twente faifi pelesentii
Female
Wachiwiri kwa Mtsogoleli wa dziko lino Saulos Chilima wati sayankhulapo kalikonse pa nkhani ya kupezeka kwa dzina lawo pa mndandanda wa omwe akuganizilidwa kuti anachita zakatangale ndi a Zunneth Sattar
Wachiwiri kwa Mtsogoleli wa dziko lino Saulosi Chilima wati sayankhulapo kalikonse pa nkhani ya kupezeka kwa dzina lawo pa mndandanda wa omwe akuganizilidwa kuti anachita zakatangale ndi a Zunefi Sata
Female
Iwo ati zisiyeni ndondomeko zonse zitsatidwe mpaka pamapeto. Chilima wakhala akuyendera zinthu zingapo ku chigawo cha mpoto
Iwo ati zisiyeni ndondomeko zonse zitsatidwe mpaka pamapeto. Chilima wakhala akuyendera zinthu zingapo ku chigawo cha mpoto
Female
pomwe akulondoloza momwe kukonzanso kwa kayendetsedwe ka zinthu mu nthambi za boma zikuyendera. A polisi amanga akuluakulu awiri omwe amatsogolela gulu lina lomwe likudzitcha mbadwa zokhudzidwa
pomwe akulondoloza momwe kukonzanso kwa kayendetsedwe ka zinthu mu nthambi za boma zikuyendera. A polisi amanga akuluakulu awiri omwe amatsogolela gulu lina lomwe likudzitcha mbadwa zokhudzidwa
Female
lomwe likufuna kuti a Martha Chizuma atule pansi udindo wawo. Awiriwa ndi a Redson Munlo komanso a Agape Khombe
lomwe likufuna kuti a Mafa Chizuma atule pansi udindo wawo. Awiriwa ndi a Redisoni Munilo komanso a Agape Khombe
Female
Gulu lomwe likudzitcha mbadwa zokhudzidwa lati mawa lachinayi likatseka ma ofesi a bungwe lothana ndi katangale la ACB kaamba koti mtsogoleli wa dziko lino Lazarus Chakwera
Gulu lomwe likudzitcha mbadwa zokhudzidwa lati mawa lachinayi likatseka ma ofesi a bungwe lothana ndi katangale la esibi kaamba koti mtsogoleli wa dziko lino Lazalasi Chakwera
Female
wakanika kuchotsa mkulu wa bungweli a Martha Chizuma. Mtsogoleli wa gululi a Redson Munlo ati afika popanga chiganizochi poona kuti a Chakwera sakuchitapo kanthu pa madandu awo
wakanika kuchotsa mkulu wa bungweli a Mafa Chizuma. Mtsogoleli wa gululi a Redisoni Muinlo ati afika popanga chiganizochi poona kuti a Chakwera sakuchitapo kanthu pa madandu awo
Female
Apolisi m'boma la Phalombe amanga a Symon Justin azaka zokwana 50 chifukwa chogwilira atsikana awiri omwe zaka zawo ndi 11 komanso 10
Apolisi m'boma la Phalombe amanga a saimoni jasitini azaka zokwana fifite chifukwa chogwilira atsikana awiri omwe zaka zawo ndi leveni komanso teni
Female
Mneneri wa police ya Phalombe a Jimmy Kapanja ati oganizilidwawa a Justin adapanga izi Ku Phalombe parish komwe atsikanawa adapita kuti akatole nkhuni
Mneneri wa police ya Phalombe a Jime Kapanja ati oganizilidwawa a Jusitini adapanga izi Ku Phalombe palishi komwe atsikanawa adapita kuti akatole nkhuni
Female
Wa chiwiri kwa nduna yowona zamalo a Deusi Gumba awuza khamu la anthu ku Mchinji kuti President Chakwera alamulira kwa zaka 10
Wa chiwiri kwa nduna yowona zamalo a Deusi Gumba awuza khamu la anthu ku Mchinji kuti Pulezidenti Chakwera alamulira kwa zaka teni
Female
A Gumba alankhura izi pa msonkhano omwe President Chakwera akupangitsa kudera la Tembwe ndipo izi zikugwirizana ndizomwe Binton Kutsaira komaso Mai Gotani Hara analankhura masiku apitawo
A Gumba alankhura izi pa msonkhano omwe Pulezidenti Chakwera akupangitsa kudera la Tembwe ndipo izi zikugwirizana ndizomwe Bintoni Kutsaira komaso Mai Gotani Hara analankhura masiku apitawo
Female
ogwira ntchito ku chipatala apezeka atafa pa nseu. Apolice m'boma la Mangochi akusakasaka anthu ena osadziwika omwe apha ogwira ntchito wa chipatala chapaboma cha Mangochi
ogwira ntchito ku chipatala apezeka atafa pa nseu. Apolisi m'boma la Mangochi akusakasaka anthu ena osadziwika omwe apha ogwira ntchito wa chipatala chapaboma cha Mangochi
Female
zi zachitika usiku wa lamulungu pa 15 May 2022 pa Malo a malonda otchedwa Soko. Ophedwayu dzinalake ndi Dinizhy Sifa
zi zachitika usiku wa lamulungu pa fifitini meyi twente twente thu pa Malo a malonda otchedwa Soko. Ophedwayu dzinalake ndi Dinize Sifa
Female
amene amachokera mmudzi mwa Lundu mfumuyaikulu Nsomba Ku Blantyre. Olankhulila police ya Mangochi sub inspector Amina Tepani Daudi watsimikizila Angaliba za nkhaniyi
amene amachokera mmudzi mwa Lundu mfumuyaikulu Nsomba Ku Bulantaya. Olankhulila polisi ya Mangochi sabu insipekita Amina Tepani Daudi watsimikizila Angaliba za nkhaniyi
Female
Apolisiwa ati akupempha onse omwe angadziwepo kanthu kuti awatsine khutu. Anthu as anu ndi mmodzi amwalira ndipo ena ambiri avulala
Apolisiwa ati akupempha onse omwe angadziwepo kanthu kuti awatsine khutu. Anthu as anu ndi mmodzi amwalira ndipo ena ambiri avulala
Female
pa ngozi ya galimoto yomwe yachitika pa Biriwiri m’boma la Ntcheu. Mkulu owona zaumoyo pa chipatala chachikulu cha Ntcheu
pa ngozi ya galimoto yomwe yachitika pa Biriwiri m’boma la Ntcheu. Mkulu owona zaumoyo pa chipatala chachikulu cha Ntcheu
Female
Dr. Steven Macheso wadzimikiza za nkhaniyi kuti alandira matupi ya anthu asanu ndi mmodzi omwe amwalilira ndi anthu ena omwe avulala Modesto nkhawa akulandira thandizo la mankhwala pa chipatala cho
Dokota Sitivini Macheso wadzimikiza za nkhaniyi kuti alandira matupi ya anthu asanu ndi mmodzi omwe amwalilira ndi anthu ena omwe avulala Modesto nkhawa akulandira thandizo la mankhwala pa chipatala cho
Female
Mneneli Police ya Ntcheu Rabecca Ndiwate wati ngoziyi yachitika pamene galimoti la mtundu wa Isuzu 400 Van, CA 9896
Mneneli Polisi ya Ntcheu Rabeka Ndiwate wati ngoziyi yachitika pamene galimoti la mtundu wa Isuzu fo handiledi vani, sie naini eiti naini sikisi
Female
linaphonya mseu ndikupita mbali y omwe kunali minibus Toyota Hiace Nambala KK8426 yomwe imayenda mbali ina ya nsewu
linaphonya mseu ndikupita mbali yomwe kunali minibasi Toyota Haisi Nambala kei kei eiti folo thu sikisi yomwe imayenda mbali ina ya nsewu
Female
Naomi Kilekwa Phiri phungu wadera la Mulanje South East, watsegulira mlatho wa Mbambazi omwe awumanga m'dera la mfumu Mulimiha
Naomi Kilekwa Phiri phungu wadera la Mulanje saufi isiti, watsegulira mlatho wa Mbambazi omwe awumanga m'dera la mfumu Mulimiha
Female
ndi ndalama zoposera 10 million kwacha za Constituency Development Fund (CDF). Polankhula pamwambo otsegulira mlathowu, a Phiri ati ndiozipereka kupitiliza kupereka zitukuko kwa anthu a dela lake
ndi ndalama zoposera teni miliyoni kwacha kwacha za konsitichuwense divelopumenti fandi (Sidiefu ). Polankhula pamwambo otsegulira mlathowu, a Phiri ati ndiozipereka kupitiliza kupereka zitukuko kwa anthu a dela lake
Female
Bwalo la milandu ku Nkhotakota la chisanu lapereka chigamulo kwa bambo Yesaya Quoto wa zaka 24 kukagwira ukaidi kwa zaka 12
Bwalo la milandu ku Nkhotakota la chisanu lapereka chigamulo kwa bambo Yesaya koto wa zaka twente folo kukagwira ukaidi kwa zaka twelofu
Female
kamba kopezeka ndi mulandu wopanga ndalama zachinyengo zama k5,000. Zokwana K575,000 pa Malo ochitira malonda a Dwangwa
kamba kopezeka ndi mulandu wopanga ndalama zachinyengo zama faifi sauzande kwacha. Zokwana faifi handiledi andi sevente faifi sauzande kwacha pa Malo ochitira malonda a Dwangwa
Female
Ana awiri awombedwa ndi galimoto ku bypass Lilongwe ndipo afela pompo. Chomwe chachitika mchakuti gulu la ana a school amachita ziwonetsero zokwiya ndikukwera kwa user fees pa school pawo
Ana awiri awombedwa ndi galimoto ku baipasi Lilongwe ndipo afela pompo. Chomwe chachitika mchakuti gulu la ana a sukulu amachita ziwonetsero zokwiya ndikukwera kwa fizi pa sukulu pawo
Female
ndipo anabwera ku nsewu komwe amawonetsa mkwiyo wawo. Galimoto yomwe yawawomba sinayime, pakali pano matupi awo anyamulidwa ndi a police
ndipo anabwera ku nsewu komwe amawonetsa mkwiyo wawo. Galimoto yomwe yawawomba sinayime, pakali pano matupi awo anyamulidwa ndi a polisi
Female
Kodi mkoyenera aBambo kupeleka mpamba wa geni kwa akazawo pomwe Iwo akungokhala pakhomo. Tumizani Maganizo anu
Kodi mkoyenera aBambo kupeleka mpamba wa geni kwa akazawo pomwe Iwo akungokhala pakhomo. Tumizani Maganizo anu
Female
A namwino omwe amagwira ntchito pa chipatala cha Queens mosalembedwa ndi boma omwe amatchedwa kuti ma upkeep ayamba kunyanyala ntchito kamba koti iwo sanalandire ndalama zawo za mwezi watha
A namwino omwe amagwira ntchito pa chipatala chakwinzi mosalembedwa ndi boma omwe amatchedwa kuti ma apukipi ayamba kunyanyala ntchito kamba koti iwo sanalandire ndalama zawo za mwezi watha
Female
Iwo ati apitiliza ntchito pokhapokha atalandira ndalama zawo, iwo ati sangapitilize kugwira ntchito pomwe a Namwino anzawo omwe analembedwa ndi boma ngati okhazikika atalandira ndalama zawo
Iwo ati apitiliza ntchito pokhapokha atalandira ndalama zawo, iwo ati sangapitilize kugwira ntchito pomwe a Namwino anzawo omwe analembedwa ndi boma ngati okhazikika atalandira ndalama zawo
Female
A Catherine chiwalo omwe ndi wankulu oyang'anila ku ward ya kungozi ati vutoli lakhuza kwambiri kagwilidwe ntchito kawo kamba koti anamwino a upkeep amathandiza kwambiri
A Cafelini chiwalo omwe ndi wankulu oyang'anila ku wadi ya kungozi ati vutoli lakhuza kwambiri kagwilidwe ntchito kawo kamba koti anamwino a apukipi amathandiza kwambiri
Female
President Lazarus Chakwera lero wafotokozera momwe zinthu ziliri mdziko muno SONA m'magawo osiyanasiyana kuphatikizapo chuma ndi zitukuko
Pulezidenti Lazalasi Chakwera lero wafotokozera momwe zinthu ziliri mdziko muno SONA m'magawo osiyanasiyana kuphatikizapo chuma ndi zitukuko
Female
Akatswiri pa nkhani za ndale, ulamuliro wabwino ndi zina akhale akutambasulira komanso kuzukuta SONA-yi pa Ndirande FM kuyambira nthawi ya 5 koloko madzulowa mu Programme ya Mutipo Chani
Akatswiri pa nkhani za ndale, ulamuliro wabwino ndi zina akhale akutambasulira komanso kuzukuta SONA-yi pa Ndirande efuemu kuyambira nthawi ya faifi koloko madzulowa mu Pulogalamu ya Mutipo Chani
Female
Bungwe lothandiza anthu mu njira zosiyanasiyana la Chimbota Community Development lati lili ndi malingaliro ofuna kupeza ndalama zomwe zithandize anthu omwe omwe akhuzidwa ndi njala m'maboma a Blantyre ndi Thyolo
Bungwe lothandiza anthu mu njira zosiyanasiyana la Chimbota komyunite divelopumenti lati lili ndi malingaliro ofuna kupeza ndalama zomwe zithandize anthu omwe omwe akhuzidwa ndi njala m'maboma a Bulantaya ndi Thyolo
Female
Ofalitsa nkhani wa bungweli, Innocent Ndala wati mwa zina, akukonza ulendo wa ndawala opezera ndalamazi omwe uchitike kuyambira pa 24 February chaka chino
Ofalitsa nkhani wa bungweli, Inosenti Ndala wati mwa zina, akukonza ulendo wa ndawala opezera ndalamazi omwe uchitike kuyambira pa twente folo febuluwale chaka chino
Female
ndipo azayenda kuchoka ku Blantyre kukafika ku Thyolo. Tikufuna tipeze ndalama zosachepera K100 Million zomwe tigwiritse ntchito pothandiza anthuwa omwe pano akukumana ndi mavuto osiyanasiyana
ndipo azayenda kuchoka ku Blantyre kukafika ku Thyolo. Tikufuna tipeze ndalama zosachepera K100 Million zomwe tigwiritse ntchito pothandiza anthuwa omwe pano akukumana ndi mavuto osiyanasiyana
Female
atero a Ndala. Pamenepo, iwo apempha anthu, kampani ndi mabungwe kuti agwirane nawo manja pozayenda nawo pa ulendowu komanso kuthandiza ndi zomwe angathe, mwa zina, kuti malingalirowa atheke
atero a Ndala. Pamenepo, iwo apempha anthu, kampani ndi mabungwe kuti agwirane nawo manja pozayenda nawo pa ulendowu komanso kuthandiza ndi zomwe angathe, mwa zina, kuti malingalirowa atheke
Female
Bungwe la chikhalidwe cha Mulhako Wa Alhomwe latsutsa malipoti oti lachotsa pa mpando a Peter Mutharika ngati patron wa bungweli
Bungwe la chikhalidwe cha Mulakho Wa Alomwe latsutsa malipoti oti lachotsa pa mpando a Pita Mutharika ngati patiloni wa bungweli
Female
Iwo akuchititsa msonkhano wa atolankhani ku Blantyre komwe adzudzula kotheratu malipoti ponena kuti zili ndi kuthekera kosokoneza anthu
Iwo akuchititsa msonkhano wa atolankhani ku Bulantaya komwe adzudzula kotheratu malipoti ponena kuti zili ndi kuthekera kosokoneza anthu.
Female
Wa pa mpando wa board ya bungweli, Muchanakwaye Mpuluka wati, patron wa bungwe lathu amasankhidwa ku msonkhano wawukulu wa pa chaka, osati ma trustee okha okha
Wa pa mpando wa bodi ya bungweli, Muchanakwaye Mpuluka wati, patiloni wa bungwe lathu amasankhidwa ku msonkhano wawukulu wa pa chaka, osati ma thilasitii okha okha
Female
ndipo mudziwenso kuti tikamachita mkumanowu mwezi wa mawa, tilibe malingaliro ofuna kuchotsa a Mutharika pa udindowu
ndipo mudziwenso kuti tikamachita mkumanowu mwezi wa mawa, tilibe malingaliro ofuna kuchotsa a Mutharika pa udindowu
Female
Iwo adzudzulanso malipoti oti bungweli lagulidwa ndi chipani china kuti lizichita zinthu mokomera icho. Ophunzira pa sukulu ya Soche Technical College ku Blantyre lero akuchita zionetsero pa sukulu yawo
Iwo adzudzulanso malipoti oti bungweli lagulidwa ndi chipani china kuti lizichita zinthu mokomera icho. Ophunzira pa sukulu ya Sochetekiniko Koleji ku Bulantaya lero akuchita zionetsero pa sukulu yawo
Female
ati zosonyeza kusakondwa ndi za kudya zomwe akumalandira. President wa bungwe loimira ophunzirawa, Edwin Huwa watiwuza kuti ayesesa kuwuza akuluakulu a sukuluyi
ati zosonyeza kusakondwa ndi za kudya zomwe akumalandira. Pulezidenti wa bungwe loimira ophunzirawa, Ediwini Huwa watiwuza kuti ayesesa kuwuza akuluakulu a sukuluyi
Female
kuti akonze vuto la chakudya chomwe akuti chikumakhala chosalongosoka koma sizikuphula kanthu. Ndirande FM yamva malipoti kuti kuchokera pomwe ophunzirawa anatsegulira pa 8 January chaka chino
kuti akonze vuto la chakudya chomwe akuti chikumakhala chosalongosoka koma sizikuphula kanthu. Ndirande efuemu yamva malipoti kuti kuchokera pomwe ophunzirawa anatsegulira pa eiti januwale chaka chino
Female
akhala akudya nsima ya ndiwo nyemba, ndipo kawiri kokha anasinthapo ndiwo ndikudyera soya pieces komanso mazira. Akuluakulu a sukuluyi sanayankhulepo kanthu pa nkhaniyi
akhala akudya nsima ya ndiwo nyemba, ndipo kawiri kokha anasinthapo ndiwo ndikudyera soya pisesi komanso mazira. Akuluakulu a sukuluyi sanayankhulepo kanthu pa nkhaniyi
Female
Yemwe anali mlangizi wa Peter Mutharika, mtsogoleri wa chipani cha DPP, Kondwani Nankhumwa wati azapikisana nawobe pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko chaka cha mawa
Yemwe anali mlangizi wa Pita Mutharika, mtsogoleri wa chipani cha Dipipi, Kondwani Nankhumwa wati azapikisana nawobe pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko chaka cha mawa
Female
A Nankhumwa ayankhula izi lero ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre, kwa nthawi yoyamba, patatha sabata chiwachotseleni mu chipanichi pamodzi ndi anthu ena ati kaamba kosowa mwambo
A Nankhumwa ayankhula izi lero ku Ndirande mu mzinda wa Bulantaya, kwa nthawi yoyamba, patatha sabata chiwachotseleni mu chipanichi pamodzi ndi anthu ena ati kaamba kosowa mwambo
Female
A Nankhumwa awuza anthu ku Ndirande-ku kuti tchutchutchu wa masomphenya ozapikisana nawo pa mpandowu afotokoza bwino lomwe mtsogolomu
A Nankhumwa awuza anthu ku Ndirande-ku kuti tchutchutchu wa masomphenya ozapikisana nawo pa mpandowu afotokoza bwino lomwe mtsogolomu
Female
Anthu osiyanasiyana kuphatikizapo achinyamata ndi amayi okhala mderali achita zinthu komanso ayimba nyimbo zosonyeza kusakondwa ndi kuchotsedwa kwa a Nankhumwa mu DPP
Anthu osiyanasiyana kuphatikizapo achinyamata ndi amayi okhala mderali achita zinthu komanso ayimba nyimbo zosonyeza kusakondwa ndi kuchotsedwa kwa a Nankhumwa mu Dipipi
Female
Anthuwa alonjezanso kuwasata a Nankhumwa kuli konse komwe angalowere pa ndale ponena kuti ndi munthu wa masomphenya
Anthuwa alonjezanso kuwasata a Nankhumwa kuli konse komwe angalowere pa ndale ponena kuti ndi munthu wa masomphenya
Female
Ku m'mawaku, Nankhumwa omwe anakhalaponso wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipanichi mchigawo cha kum'mwera, anali nawo ku mwambo wa mapemphero olandira m'busa Alex Ngwaya ku Makata CCAP
Ku m'mawaku, Nankhumwa omwe anakhalaponso wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipanichi mchigawo cha kum'mwera, anali nawo ku mwambo wa mapemphero olandira m'busa Alekisi Ngwaya ku Makata Sisiepi
Female
Mafumu ena a chilhomwe ati akutsutsana ndi ganizo la boma lozodza Senior Chief Kaduya kukhala mfumu yayikulu (paramount chief) ya alhomwe
Mafumu ena a chilomwe ati akutsutsana ndi ganizo la boma lodzoza Siniyo Tchifi Kaduya kukhala mfumu yayikulu (Palamaunti Tchifi ) ya alomwe
Female
Iwo akuchititsa msonkhano wa atolankhani kwa T/A Ngolongoliwa m'boma la Thyolo komwe akuti boma silinatsatire bwino mbiri pomwe limasankha a Kaduya kukhala pa mpandowu
Iwo akuchititsa msonkhano wa atolankhani kwa Tie Ngolongoliwa m'boma la Thyolo komwe akuti boma silinatsatire bwino mbiri pomwe limasankha a Kaduya kukhala pa mpandowu
Female
Motsogozedwa ndi mfumu Nkhulambe ya ku Phalombe komanso mfumu Ndalama ya ku Thyolo, mafumuwa adzudzulanso akuluakulu a bungwe lawo la Mulhako Wa Alhomwe kaamba kosawunikira mozama pa kasankhidwe ka mfumuyi
Motsogozedwa ndi mfumu Nkhulambe ya ku Phalombe komanso mfumu Ndalama ya ku Thyolo, mafumuwa adzudzulanso akuluakulu a bungwe lawo la Mulakko Wa Alomwe kaamba kosawunikira mozama pa kasankhidwe ka mfumuyi
Female
Iwo ati phata la a Kaduya ndi la mtundu wa a Mang'anja osati alhomwe, choncho iwo akufuna akhalenso ndi mfumu yawo yayikulu
Iwo ati phata la a Kaduya ndi la mtundu wa a Mang'anja osati alomwe, choncho iwo akufuna akhalenso ndi mfumu yawo yayikulu
Female
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera wakhazikitsa a Kaduya pa mpandowu dzulo m'boma la Phalombe
Mtsogoleri wa dziko lino, Dokota Lazalasi Chakwera wakhazikitsa a Kaduya pa mpandowu dzulo m'boma la Phalombe
Female
Gulu la alakatuli ena mdziko muno lati liri ndi malingaliro ofuna kuthandiza ophunzira a form 4 a msukulu za secondary zosiyanasiyana omwe ali pa chiopsezo chosalemba nawo mayeso a MANEB kaamba ka mavuto a za chuma
Gulu la alakatuli ena mdziko muno lati liri ndi malingaliro ofuna kuthandiza ophunzira a fomu folo a msukulu za sekondale zosiyanasiyana omwe ali pa chiopsezo chosalemba nawo mayeso a MANEBU kaamba ka mavuto a za chuma.
Female
Gululi lati lati lichititsa chiphwando cha ndakatulo lero madzulo ku Mibawa Multipurpose Hall mu mzinda wa Blantyre
Gululi lati lati lichititsa chiphwando cha ndakatulo lero madzulo ku Mibawa Matipeposi holo mu mzinda wa Bulantaya
Female
komwe malingaliro ndi ofuna kupeza ndalama zosachepera K2 Million zomwe zithandize ophunzira 1,000
komwe malingaliro ndi ofuna kupeza ndalama zosachepera thu miliyoni kwacha zomwe zithandize ophunzira wani sauzande
Female
Chiphwandochi chikutsatira malipoti a posachedwapa omwe ati ophunzira opitilira 29 thousand alephera kulemba nawo mayeso kaamba ka mavuto a za chuma
Chiphwandochi chikutsatira malipoti a posachedwapa omwe ati ophunzira opitilira 2twente naini sauzande alephera kulemba nawo mayeso kaamba ka mavuto a za chuma
Female
M'modzi mwa alakatuliwa, Hudson Chamasowa watiwuza kuti ndi zosamveka kuti ophunzirawa alephere kulemba mayeso a MANEB kaamba ka mavuto a za chuma, ndipo ndi chifukwa aganiza zothandizapo
M'modzi mwa alakatuliwa, Hadisoni Chamasowa watiwuza kuti ndi zosamveka kuti ophunzirawa alephere kulemba mayeso a MANEBU kaamba ka mavuto a za chuma, ndipo ndi chifukwa aganiza zothandizapo
Female
Ena mwa alakatuli omwe akalakatule ku chiphwandochi ndi Amfumu Kenneth Khondiwa, Deus Sandram, Raphael Sitima komanso Aisha Samson
Ena mwa alakatuli omwe akalakatule ku chiphwandochi ndi Amfumu Kenefi Khondiwa, Deyasi Sandiramu, Rafaelo Sitima komanso Aisha Samisoni
Female
Bungwe logulitsa magetsi la ESCOM lati lakumana ndi vuto la kuzima kwa makina ake zomwe zachititsa kuti madera ochuluka mdziko muno akhale opanda magetsi
Bungwe logulitsa magetsi la esikomu lati lakumana ndi vuto la kuzima kwa makina ake zomwe zachititsa kuti madera ochuluka mdziko muno akhale opanda magetsi
Female
Makinawa, malingana ndi ESCOM, azima nthawi ya Quarter to thu masanawa ndipo kafukufuku ofuna kupeza gwero la izi, ali mkati
Makinawa, malingana ndi esikomu, azima nthawi ya kota tu thu masanawa ndipo kafukufuku ofuna kupeza gwero la izi, ali mkati
Female
Akuluakulu ena a chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive-DPP akuchititsa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Blantyre
Akuluakulu ena a chipani chotsutsa boma cha Demokilatiki pulogilesivi-Dipipi akuchititsa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Bulantaya
Female
Mwa zina, iwo akuyankhapo pa zomwe mlangizi wa mtsogoleri wa chipanichi, a Kondwani Nankhumwa wayankhula kuti akuluakulu ku chipanichi
Mwa zina, iwo akuyankhapo pa zomwe mlangizi wa mtsogoleri wa chipanichi, a Kondwani Nankhumwa wayankhula kuti akuluakulu ku chipanichi
Female
akufuna kusintha nthumwi zopita ku msonkhano wawukulu chaka cha mawa. Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipanichi mchigawo cha kum'mwera, George Chaponda komano mneneri wa DPP, Shadric Namalomba ndi ena mwa anthu omwe akuyankhula
akufuna kusintha nthumwi zopita ku msonkhano wawukulu chaka cha mawa. Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipanichi mchigawo cha kum'mwera, Joji Chaponda komano mneneri wa Dipipi, Shadileki Namalomba ndi ena mwa anthu omwe akuyankhula
Female
Mchipani cha DPP mwakhala muli kukokanakokana kuchokera pomwe chinachoka m'boma mchaka cha 2020. Msangalatsi wina (DJ) okhala mu mzinda wa Liverpool ku England
Mchipani cha Dipipi mwakhala muli kukokanakokana kuchokera pomwe chinachoka m'boma mchaka cha twente twente. Msangalatsi wina (Dijeyi) okhala mu mzinda wa Livapu ku Ingilandi
Female
Charity Saiwala yemwe amadziwika ndi dzina loti DJ Chaz Grooving wapereka thandizo la katundu osiyanasiyana kwa anthu omwe anakhuzidwa ndi namondwe wa Freddy
Tchalite Saiwala yemwe amadziwika ndi dzina loti Dijeyi Tchazi Guluving’izi wapereka thandizo la katundu osiyanasiyana kwa anthu omwe anakhuzidwa ndi namondwe wa Fulede
Female
miyezi yapitayo ku Soche mu mzinda wa Blantyre. Thandizoli lomwe ndi la ndalama zopitilira K500 thousand
miyezi yapitayo ku Soche mu mzinda wa Bulantaya. Thandizoli lomwe ndi la ndalama zopitilira faifi handiledi sauzande
Female