audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
laperekedwa ngati mbali imodzi ya chisangalalo cha kubadwa kwa Yesu, malingana ndi chipembezi cha chikhristu. Pali anthu ena akufuna kusangalala Koma kuthekera alibe chifukwa anakhuzika ndi namondwe uja
laperekedwa ngati mbali imodzi ya chisangalalo cha kubadwa kwa Yesu, malingana ndi chipembezi cha chikhrisitu. Pali anthu ena akufuna kusangalala Koma kuthekera alibe chifukwa anakhuzika ndi namondwe uja
Female
Ndiye ineyo ndangothandizapo ena mwa iwo kuti tisangalale limodzi, watero Sayiwala poyankhula nafe kuchokera mu mzinda wa Liverpool
Ndiye ineyo ndangothandizapo ena mwa iwo kuti tisangalale limodzi, watero Sayiwala poyankhula nafe kuchokera mu mzinda wa Livapu
Female
Kuno ku mudzi, mayiyu DJ Chaz Grooving anayimililidwa ndi mtolankhani wina, Andrew Magombo. Zokonzekera zonse zokhuza kuwonetsa kanema wina yemwe mutu wake ndi Is the president dead
Kuno ku mudzi, mayiyu Dijeyi Tchazi Guluving’izi anayimililidwa ndi mtolankhani wina, Andulu Magombo. Zokonzekera zonse zokhuza kuwonetsa kanema wina yemwe mutu wake ndi izi ve pulezidenti dedi
Female
akuti zili mchimake kuti iwonetsedwe mu mzinda wa Blantyre, mawa loweruka. Isaac Misoya yemwe ndi m'modzi mwa anthu omwe ajambula nawo kanemayu
akuti zili mchimake kuti iwonetsedwe mu mzinda wa Bulantaya, mawa loweruka. Aizeki Misoya yemwe ndi m'modzi mwa anthu omwe ajambula nawo kanemayu
Female
watiwuza posachedwapa kuti zosamwitsa zomwe anakumana nazo powonetsa kanema yemweyu mu mzinda wa Lilongwe kumayambilira a mwezi uno, zakonzedwa
watiwuza posachedwapa kuti zosamwitsa zomwe anakumana nazo powonetsa kanema yemweyu mu mzinda wa Lilongwe kumayambilira a mwezi uno, zakonzedwa
Female
Mu mzinda wa Lilongwe, kanemayu anali ndi magawo ena omwe samanveka mawu powoneka zomwe zinakwiyitsa anthu a mu mzindawu, koma a Misoya ati anthu a ku Blantyre akasangalala naye
Mu mzinda wa Lilongwe, kanemayu anali ndi magawo ena omwe samanveka mawu powoneka zomwe zinakwiyitsa anthu a mu mzindawu, koma a Misoya ati anthu a ku Bulantaya akasangalala naye
Female
Takonza mavuto omwe tinali nawo poyamba paja. Anthu awonera ndithu kanema yense bwinobwino, atero a Misoya
Takonza mavuto omwe tinali nawo poyamba paja. Anthu awonera ndithu kanema yense bwinobwino, atero a Misoya
Female
Pamenepa, iwo apempha anthu kuti abwere mwawunyinji ku Amaryllis Hotel komwe akayankhidwe funso la ngati president Wamwalira kapena ayi, malingana ndi kanemayu
Pamenepa, iwo apempha anthu kuti abwere mwawunyinji ku Amalezi hotelo komwe akayankhidwe funso la ngati pulezidenti Wamwalira kapena ayi, malingana ndi kanemayu
Female
Bwalo la milandu yokhuza ndalama mu mzinda wa Lilongwe lizapitilira kumva mlandu okhuza kampani ya bus ya National Bus Services pa 5 ndi pa 6 February chaka cha m'mawa
Bwalo la milandu yokhuza ndalama mu mzinda wa Lilongwe lizapitilira kumva mlandu okhuza kampani ya basi ya Neshono basi sevisezi pa faifi ndi pa sikisi febuluwale chaka cha m'mawa
Female
Iyitu ndi nkhani yomwe mlangizi wa boma pa za malamulo, a Thabo Chakaka Nyirenda anasumira kampaniyi pa momwe inatengera ndi kumayendetsa ntchito za malo okwelera bus mmizinda ya dziko lino
Iyitu ndi nkhani yomwe mlangizi wa boma pa za malamulo, a Thabo Chakaka Nyirenda anasumira kampaniyi pa momwe inatengera ndi kumayendetsa ntchito za malo okwelera basi mmizinda ya dziko lino
Female
Posachedwapa, kampaniyi kudzera mwa wa pa mpando wake yemwe ndi odziwika bwino pa ntchito za malonda, Leston Mulli waperekera umboni wa kalata zofotokoza momwe anatengera malowa
Posachedwapa, kampaniyi kudzera mwa wa pa mpando wake yemwe ndi odziwika bwino pa ntchito za malonda, Lesitoni Muli waperekera umboni wa kalata zofotokoza momwe anatengera malowa
Female
omwe a Chakaka Nyirenda akuti panali kusasata malamulo. Lawyer wa a Mulli, John Kalampa wati kalata zomwe aperekazi
omwe a Chakaka Nyirenda akuti panali kusasata malamulo. Loya wa a Muli, Joni Kalampa wati kalata zomwe aperekazi
Female
zomwe mwa zina ndi yochoka ku ofesi ya Public Private Partnership Commission (PPPC), zinawalola kutenga malowa pomwe amagula kampani ya Shire Bus Lines pofuna kuwonetsetsa kuti akupeza phindu
zomwe mwa zina ndi yochoka ku ofesi ya pabuliki pulaiveti patinashipi komishoni (pipipisi), zinawalola kutenga malowa pomwe amagula kampani ya Shire Basi Layinzi pofuna kuwonetsetsa kuti akupeza phindu
Female
Amayi ogwira ntchito ku bungwe lopopa ndi kugulitsa madzi la Blantyre Water Board lapereka mphatso zosiyanasiyana
Amayi ogwira ntchito ku bungwe lopopa ndi kugulitsa madzi la Bulantaya wota bodi lapereka mphatso zosiyanasiyana
Female
kwa amayi omwe angobereka kumene pa zipatala za Limbe ndi Ndirande mu mzinda wa Blantyre. Amayiwa ati achita izi ngati mbali imodzi ya chikondwelero cha kubadwa kwa Ambuye Yesu
kwa amayi omwe angobereka kumene pa zipatala za Limbe ndi Ndirande mu mzinda wa Bulantaya. Amayiwa ati achita izi ngati mbali imodzi ya chikondwelero cha kubadwa kwa Ambuye Yesu
Female
chomwe akhristu amachita pa 25 December chaka chilichonse. M'modzi mwa amayiwa, mayi Lena Misiri omwe anayimilira mkulu wa zolemba anthu ku Blantyre water boeard
chomwe akhrisitu amachita pa twente faifi Disemba chaka chilichonse. M'modzi mwa amayiwa, mayi Lena Misiri omwe anayimilira mkulu wa zolemba anthu ku Bulantaya wota bodi
Female
ati anthu omwe ali mzipatalazi ndi makasitomala awo choncho anachiwona cha mnzeru kuwayendera mu nyengo ino. Bungweli lapereka sugar, zokumwa, soap ndi mabigiri, mwa zina, mzipatalazi
ati anthu omwe ali mzipatalazi ndi makasitomala awo choncho anachiwona cha mnzeru kuwayendera mu nyengo ino. Bungweli lapereka shuga, zokumwa, sopo ndi mabigiri, mwa zina, mzipatalazi
Female
Ndipo m'mawu ake, m'modzi mwa amayi omwe alandira mphatsoyi omwe abadwitsa mwana dzulo pa chipatala cha Ndirande, mayi Jessie Mpaweni athokoza Blantyre water board kaamba ka thandizoli
Ndipo m'mawu ake, m'modzi mwa amayi omwe alandira mphatsoyi omwe abadwitsa mwana dzulo pa chipatala cha Ndirande, mayi Jese Mpaweni athokoza Bulantaya wota bodi kaamba ka thandizoli
Female
Mkulu wina wochita malonda, Alvis Matiki yemwe amakhala mdziko la South Africa wapereka mipira ya ndalama pafupifupi K1.6 Million ku team ya mpira wa miyendo ya Ndirande Stars
Mkulu wina wochita malonda, Avisi Matiki yemwe amakhala mdziko la saufi afilika wapereka mipira ya ndalama pafupifupi wani pointi sikisi miliyoni kwacha ku timu ya mpira wa miyendo ya Ndirande Sitazi
Female
Timuyi, yomwe imasewera mu ligi ya chigawo cha kum'mwera ya Thumbs up, yalandira thandizoli patsogolo pa masewero a kamuthemuthe ofuna kuzipezera malo mu TNM Super League omwe akubwera posachedwapa
Timuyi, yomwe imasewera mu ligi ya chigawo cha kum'mwera ya fambuzi apu, yalandira thandizoli patsogolo pa masewero a kamuthemuthe ofuna kuzipezera malo mu Tieniemu supa ligi omwe akubwera posachedwapa
Female
Ndipo m'mawu ake, mkulu oyendetsa ntchito za timuyi, Kulua Ngwira wati ali ndi chimwemwe kaamba ka thandizoli ndipo wapempha anthu enanso akufuna kwabwino kuti agwepo ndi kuthandiza Ndirande Stars
Ndipo m'mawu ake, mkulu oyendetsa ntchito za timuyi, Kulua Ngwira wati ali ndi chimwemwe kaamba ka thandizoli ndipo wapempha anthu enanso akufuna kwabwino kuti agwepo ndi kuthandiza Ndirande Sitazi
Female
Timu yathu ikufunikira zambiri moti thandizo ilili lichepesa ena mwa mavuto athu, atero a Ngwira
Timu yathu ikufunikira zambiri moti thandizo ilili lichepesa ena mwa mavuto athu, atero a Ngwira
Female
A Walter Nyamilandu Manda agonja pa chisankho cha President ku bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo mdziko muno
A Wota Nyamilandu Manda agonja pa chisankho cha Pulezidenti ku bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo mdziko muno
Female
Iwo agonjetsedwa ndi a Fleetwood Haiya ndi mavoti 23 ku 13 pa chisankho chomwe chachitika mu mzinda wa Mzuzu komwe bungweli likuchititsa msonkhano wake osankha adindo
Iwo agonjetsedwa ndi a Fulitihudu Haiya ndi mavoti twente fili ku fetini pa chisankho chomwe chachitika mu mzinda wa Mzuzu komwe bungweli likuchititsa msonkhano wake osankha adindo
Female
Nthumwi ku msonkhanowu zasankhanso a Madalitso Kuyera kukhala wachiwiri oyamba kwa a Haiya pomwe Dr Lameck Zetu Khonje asankhidwa kukhala wachiwiri wa wachiwiri wa a Haiya
Nthumwi ku msonkhanowu zasankhanso a Madalitso Kuyera kukhala wachiwiri oyamba kwa a Haiya pomwe Dokota Lameki Zetu Khonje asankhidwa kukhala wachiwiri wa wachiwiri wa a Haiya
Female
Mayi Fellistus Dossi asankhidwa kukhala oyimira amayi ku bungweli pomwe a Daud Nthanthiko, a Chimango Munthali, a Patrick Kapanga komanso a Benard Harawa asankhidwa kukhala mamembala a komiti yayikulu ku bungwe la FAM
Mayi Felisitasi Dosi asankhidwa kukhala oyimira amayi ku bungweli pomwe a Daudi Nthanthiko, a Chimango Munthali, a Patiliki Kapanga komanso a Benadi Harawa asankhidwa kukhala mamembala a komiti yayikulu ku bungwe la FAMU
Female
Kampani yopanga mankhwala kuchokera ku zomera ya Africa Herbal Mixture yadandawula kaamba ka kuchedwa kwa bungwe loona za mankhwala la Pharmacy and Medicines Regulatory Authority-PMRA
Kampani yopanga mankhwala kuchokera ku zomera ya Afulikani Hebo Mikisicha yadandawula kaamba ka kuchedwa kwa bungwe loona za mankhwala la Famase andi medisinzi legyuletale ofolite - piemualae
Female
kuvomereza mauthenga ochemelera mankhwala ake pa wailesi ndi kanema. Malingana ndi mkulu wa kampaniyi, Joel Chirambo
kuvomereza mauthenga ochemelera mankhwala ake pa wailesi ndi kanema. Malingana ndi mkulu wa kampaniyi, Jowelo Chirambo
Female
kampani yawo inasatira zonse zofunikira kukwanilitsa, mauthenga a mankhwala otere asanayambe kuwulutsidwa pa pa wailesi
kampani yawo inasatira zonse zofunikira kukwanilitsa, mauthenga a mankhwala otere asanayambe kuwulutsidwa pa pa wailesi
Female
Pamenepa, a Chirambo apempha PMRA ifulumizitse kuwayankha pa mauthenga omwe anapereka, ponena kuti chidodo chomwe chilipo chikukhudza ntchito za malonda awo
Pamenepa, a Chirambo apempha Piemualae ifulumizitse kuwayankha pa mauthenga omwe anapereka, ponena kuti chidodo chomwe chilipo chikukhudza ntchito za malonda awo
Female
Sitinakwanitsa kuyankhula ndi mneneri wa PMRA, a Joseph Josiah omwe samayankha lamya yawo ya m'manja titawayimbira
Sitinakwanitsa kuyankhula ndi mneneri wa Piemualae, a Jozefe Josiya omwe samayankha lamya yawo ya m'manja titawayimbira
Female
M'mwezi wa June chaka chino, abungwe a PMRA komanso Malawi Communications Regulatory Authority-MACRA analengeza kuti mauthenga onse okhuza mankhwala a zisamba
M'mwezi wa Juni chaka chino, abungwe a Piemualae komanso Malawi komyunikeshonzi legyletale ofolite-MAKILA analengeza kuti mauthenga onse okhuza mankhwala a zisamba
Female
aziyamba kaye awawunika asanayambe kulengezedwa pa wailesi ndi pa kanema, monga mwa malamulo. Apolisi mu mzinda wa Blantyre amanga khansala wa chipani cha Democratic Progressive-DPP
aziyamba kaye awawunika asanayambe kulengezedwa pa wailesi ndi pa kanema, monga mwa malamulo. Apolisi mu mzinda wa Blulantaya amanga khansala wa chipani che Demokilatiki pulogilesivi-Dipiipi
Female
wa ward ya Soche East mu mzindawu, Leonard Chimbanga pomuganizira kuti wapezeka ndi mfuti popanda kalata zomuyenereza kutero
wa wadi ya Soche isiti mu mzindawu, Leonadi Chimbanga pomuganizira kuti wapezeka ndi mfuti popanda kalata zomuyenereza kutero
Female
Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi ku chigawo cha kum'mwera cha kumadzulo, Beatrice Mikuwa watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati a Chimbanga
Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi ku chigawo cha kum'mwera cha kumadzulo, Bitilisi Mikuwa watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati a Chimbanga
Female
atengeledwa ku bwalo la milandu posachedwapa. Iwo akusungidwa ku polisi ya Chileka, ku Blantyre komweko. Chipani chotsutsa boma Cha Democratic Progressive-DPP
atengeledwa ku bwalo la milandu posachedwapa. Iwo akusungidwa ku polisi ya Chileka, ku Bulantaya komweko. Chipani chotsutsa boma Cha DemoDemokilatiki Pulogilesivi-Dipipi
Female
chasankha a Grezelder Jeffrey kukhala wachiwiri kwa mtsogoleri wake mchigawo cha pakati. Kalata yomwe a mtsogoleri wa chipanichi, Peter Mutharika watulutsa
chasankha a Gilezeda Jefule kukhala wachiwiri kwa mtsogoleri wake mchigawo cha pakati. Kalata yomwe a mtsogoleri wa chipanichi, Pita Mutharika watulutsa
Female
yati udindo wa a Jeffrey omwe unali Mlembi wamkulu tsopano ukhala m'manja mwa Dr. Clement Mwale. Gulu la chikhalidwe la Mulhako wa Alhomwe lalengeza kuti lapeza thandizo la ndalama zokwana K46 Million
yati udindo wa a Jefule omwe unali Mlembi wamkulu tsopano ukhala m'manja mwa Dokota Kilementi Mwale. Gulu la chikhalidwe la Mulako wa Alomwe lalengeza kuti lapeza thandizo la ndalama zokwana fote sikisi miliyoni
Female
kuchokera ku bungwe la Cultural Emergency Response la ku Netherlands. Mkulu wa gulu la Mulhako wa Alhomwe, Pius Mvenya watiwuza lero kuti thandizoli
kuchokera ku bungwe la kachulo imejese lisiposi la ku Nefelanzis. Mkulu wa gulu la Mulakho wa Alomwe, Piyasi Mvenya watiwuza lero kuti thandizoli
Female
ligwira ntchito yofukula mbiri ya chikhalidwe cha chilhomwe, kumangira nyumba ya zosunga mizimu zotchedwa mlukunuwa kwa Chonde ku Mulanje komanso kubzala mitengo
ligwira ntchito yofukula mbiri ya chikhalidwe cha chilomwe, kumangira nyumba ya zosunga mizimu zotchedwa mlukunuwa kwa Chonde ku Mulanje komanso kubzala mitengo
Female
yomwe mwa ina mwa iyo izithandizira pa mankhwala achikuda. Malingana ndi a Mvenya, zinthu zambiri zokhuza chikhalidwe kuphatikiza mikoko yogona
yomwe mwa ina mwa iyo izithandizira pa mankhwala achikuda. Malingana ndi a Mvenya, zinthu zambiri zokhuza chikhalidwe kuphatikiza mikoko yogona
Female
inatayika pomwe namondwe wa Freddy anaomba ena mwa anthu koma ndi thandizoli akukhulupilira kuti zambiri zibwelera mchimake
inatayika pomwe namondwe wa Fulede anaomba ena mwa anthu koma ndi thandizoli akukhulupilira kuti zambiri zibwelera mchimake
Female
Bungwe la Chimbota Community Development lati lipitilira kuthandiza anthu osiyanasiyana ndi chakudya pomwe madera ambiri akukumana ndi vuto la njala
Bungwe la Chimbota komyunite divelopumenti lati lipitilira kuthandiza anthu osiyanasiyana ndi chakudya pomwe madera ambiri akukumana ndi vuto la njala
Female
Mkulu wa bungweli, Kevin Troughton watiwuza kuti pakadali pano, bungwe lawo lafikira anthu opitilira 500, ena mwa iwo okalamba, ndi thandizo lotere
Mkulu wa bungweli, Kevini Thilautoni watiwuza kuti pakadali pano, bungwe lawo lafikira anthu opitilira faifi handiledi, ena mwa iwo okalamba, ndi thandizo lotere
Female
ndipo ali ndi chikhulupiliro kuti lithandiza kusintha miyoyo yawo. Bungwe la Chimbota Community Development likupereka chimanga kwa anthuwa chomwe thandizo la ndalama zake zina zachokera ku bungwe la ku Ireland la Africa Direct
ndipo ali ndi chikhulupiliro kuti lithandiza kusintha miyoyo yawo. Bungwe la Chimbota komyunite divelopumenti likupereka chimanga kwa anthuwa chomwe thandizo la ndalama zake zina zachokera ku bungwe la ku ailandi la Afulika dailekiti
Female
Ena mwa Madera omwe afikilidwa ndi a Ndirande ndi Machinjiri mu mzinda wa Blantyre. Nthambi ya achinyamata ku bungwe la oyimba la Musician Union of Malawi (MUM)
Ena mwa Madera omwe afikilidwa ndi a Ndirande ndi Machinjiri mu mzinda wa Bulantaya. Nthambi ya achinyamata ku bungwe la oyimba la Myuzishani yuniyoni ofu Malawi (MUMU)
Female
yasankha mwini wake wa kampani ya Choice Construction, a Daniel Makaula kukhala mlangizi wake. Kalata yomwe nthambiyi yatulutsa ndipo wasainira ndi mlembi wake, Ruth Ngugwe
yasankha mwini wake wa kampani ya Tchoisi konsitilakishoni, a Daniele Makaula kukhala mlangizi wake. Kalata yomwe nthambiyi yatulutsa ndipo wasainira ndi mlembi wake, Rufi Ngugwe
Female
yati nthambiyi yasankha a Makaula kaamba ka chidwi chawo potukula mayimbidwe mdziko muno. A Makaula, omwe avomera udindowu wa mlangiziwu, agwira ntchito kwa zaka ziwiri
yati nthambiyi yasankha a Makaula kaamba ka chidwi chawo potukula mayimbidwe mdziko muno. A Makaula, omwe avomera udindowu wa mlangiziwu, agwira ntchito kwa zaka ziwiri
Female
Apolisi atseka msewu olunjika ku Sanjika palace ndi galimoto ya Nyala (trooper) pomwe ochita zionetsero zodana ndi boma la mgwirizano wa Tonse akuyandikira kufika pa mphambano ya msewuwu
Apolisi atseka msewu olunjika ku Sanjika palesi ndi galimoto ya Nyala (thulupa) pomwe ochita zionetsero zodana ndi boma la mgwirizano wa Tonse akuyandikira kufika pa mphambano ya msewuwu
Female
Iwo, pansi pa gulu lomenyera ufulu la Malawi First, akupita ku ofesi za khonsolo ya boma la Blantyre kukasiya kalata za madandawulo awo. Anthu osiyanasiyana akutenga nawo mbali pa zionetserozi
Iwo, pansi pa gulu lomenyera ufulu la Malawi Fesiti, akupita ku ofesi za khonsolo ya boma la Bulantaya kukasiya kalata za madandawulo awo. Anthu osiyanasiyana akutenga nawo mbali pa zionetserozi
Female
Gulu lina lomenyera ufulu wa anthu la Malawi First, lero likuchititsa zionetsero mu mzinda wa Blantyre zomwe cholinga chake ndi kusonyeza kusakondwa ndi boma la mgwirizano wa Tonse
Gulu lina lomenyera ufulu wa anthu la Malawi Fesiti, lero likuchititsa zionetsero mu mzinda wa Bulantaya zomwe cholinga chake ndi kusonyeza kusakondwa ndi boma la mgwirizano wa Tonse
Female
Gululi, lomwe likutsogozedwa ndi a Bon Kalindo, likuti mavuto a za chuma ndi zina achuluka ndipo akufuna adindo achitepo kanthu, kulephera kutero, president Lazarus Chakwera atule pansi udindo
Gululi, lomwe likutsogozedwa ndi a Boni Kalindo, likuti mavuto a za chuma ndi zina achuluka ndipo akufuna adindo achitepo kanthu, kulephera kutero, pulezidenti Lazalasi Chakwera atule pansi udindo
Female
Iwo akasiya kalata za nkhawa zawo ku ofesi ya khonsolo ya boma la Blantyre. Anthu osiyanasiyana ambiri mwa Iwo achinyamata ndi omwe akuchita nawo zionetserozi
Iwo akasiya kalata za nkhawa zawo ku ofesi ya khonsolo ya boma la Bulantaya. Anthu osiyanasiyana ambiri mwa Iwo achinyamata ndi omwe akuchita nawo zionetserozi
Female
Nduna ya zofalitsa nkhani, Moses Kunkuyu yayamikira ntchito zosiyanasiyana zolimbikitsa chitukuko zomwe atolankhani mdziko muno amakhala akugwira
Nduna ya zofalitsa nkhani, Mozesi Kunkuyu yayamikira ntchito zosiyanasiyana zolimbikitsa chitukuko zomwe atolankhani mdziko muno amakhala akugwira
Female
Iwo ayankhula izi lero ku Mulanje pa msonkhano wawukulu wa pa chaka komanso osankha adindo omwe bungwe la atolankhani la Blantyre Press Club-BPC lachititsa lero
Iwo ayankhula izi lero ku Mulanje pa msonkhano wawukulu wa pa chaka komanso osankha adindo omwe bungwe la atolankhani la Bulantaya pulesi kilabu-Bipisi lachititsa lero
Female
Malingana ndi a Kunkuyu, dziko silingayende bwino ngati atolankhani sakugwira ntchito yawo moyenelera ndipo wapempha kuti asamatenge mbali polemba, kutsindikiza komanso kuwulutsa nkhani zawo
Malingana ndi a Kunkuyu, dziko silingayende bwino ngati atolankhani sakugwira ntchito yawo moyenelera ndipo wapempha kuti asamatenge mbali polemba, kutsindikiza komanso kuwulutsa nkhani zawo
Female
Pa msonkhano wawukuluwu, atolankhani a BPC-wa asankha adindo atsopano motere: Bungwe la Forum for Democracy and Rights Defenders-FDRD
Pa msonkhano wawukuluwu, atolankhani a Bipisi-wa asankha adindo atsopano motere: Bungwe la folamu fo demokilase andi laitsi difendazi-efudialadi
Female
lero likutsogolera anthu pa ulendo wa ndawala omwe cholinga chake ndi kusonyeza kusakondwa ndi nkhondo yomwe ikuchitika pakati pa mayiko a Israel ndi Palestine
lero likutsogolera anthu pa ulendo wa ndawala omwe cholinga chake ndi kusonyeza kusakondwa ndi nkhondo yomwe ikuchitika pakati pa mayiko a Izilaeli ndi Palesitini
Female
Bungwe liyenda kuchokera pa Kamuzu Upper stadium kukafika pa Ginnery Corner kenako kubweleranso pa Kamuzu Upper Stadium
Bungwe liyenda kuchokera pa Kamuzu apa sitediyamu kukafika pa Jinale kona kenako kubweleranso pa Kamuzu apa sitediyamu
Female
Pakadali pano, apolisi ndi anthu ena afika kale pa malo onyamukira ulendowu. Timu ya mpira wa manja ya dziko lino ya Queens
Pakadali pano, apolisi ndi anthu ena afika kale pa malo onyamukira ulendowu. Timu ya mpira wa manja ya dziko lino ya Kwinzi
Female
yagonja masewero atatu omwe yasewera mosatana ku mpikisano wa Fast 5 omwe ukuchitikira ku New Zealand
yagonja masewero atatu omwe yasewera mosatana ku mpikisano wa Fasiti faifi omwe ukuchitikira ku Nyuzilandi
Female
Timu ya mpira wa manja ya dziko linoyi yasewera masewero ake m'bandakucha wa lero. Matimu omwe agonjetsa Queens ndi News Zealand ndi ma basket 42 kwa 13
Timu ya mpira wa manja ya dziko linoyi yasewera masewero ake m'bandakucha wa lero. Matimu omwe agonjetsa kwinzi ndi nyuzilandi ndi ma basiketi fotethu kwa fetini
Female
Jamaica ndi ma basket 41 ku 37 komanso England ndi ma basket 41 kwa 30. Bambo wa zaka 43, Steve Phiri ali mchitokosi cha apolisi ku Lilongwe
Jamaika ndi ma basiketi fotewani ku feteseveni komanso Ingilandi ndi ma basiketi fotewani kwa fete. Bambo wa zaka fotefili, Sitivini Phiri ali mchitokosi cha apolisi ku Lilongwe
Female
pomuganizira kuti amabera anthu katundu ndi ndalama ponamizira kuti ndi oyendetsa galimoto yonyamula anthu (taxi). Ofalitsa nkhani ku polisi ya Lilongwe, Hastings Chigalu
pomuganizira kuti amabera anthu katundu ndi ndalama ponamizira kuti ndi oyendetsa galimoto yonyamula anthu (takisi). Ofalitsa nkhani ku polisi ya Lilongwe, Hesiting’izi Chigalu
Female
wati apolisi akufunafunanso anthu ena atatu omwe akuwaganizira kuti anapalamula nawo mlanduwu. Malipoti akuti oganizilidwawa
wati apolisi akufunafunanso anthu ena atatu omwe akuwaganizira kuti anapalamula nawo mlanduwu. Malipoti akuti oganizilidwawa
Female
anachitira chiwembu mkulu wina yemwe anakwera galimoto yawo ndipo anamubera lamya za mtundu wa Iphone komanso laptop ndipo zonse ndi za ndalama zokwana K5.2 Million
anachitira chiwembu mkulu wina yemwe anakwera galimoto yawo ndipo anamubera lamya za mtundu wa aifoni komanso laputopu ndipo zonse ndi za ndalama zokwana faifi pointu thu miliyoni kwacha
Female
Kafukufuku wa apolisi wapeza ziphatso za umzika ndi Zina zoyendetsera galimoto ku nyumba kwa oganizilidwawa
Kafukufuku wa apolisi wapeza ziphatso za umzika ndi Zina zoyendetsera galimoto ku nyumba kwa oganizilidwawa
Female
Anthu osiyanasiyana kudzera masamba a mchezo awonetsa kukhumudwa ndi kugwetsedwa kwa mphanvu ya ndalama ya kwacha ndi banki yayikulu ya dziko muno, ya Reserve
Anthu osiyanasiyana kudzera masamba a mchezo awonetsa kukhumudwa ndi kugwetsedwa kwa mphanvu ya ndalama ya kwacha ndi banki yayikulu ya dziko muno, ya lizevu
Female
Ndalamayi yagwa ndi K44 pa K100 iliyonse. Kalata yomwe bankiyi yatulutsa, ikuonetsa kuti izi zachitika pofuna kuthandizira kupezeka kwa ndalama za kunja
Ndalamayi yagwa ndi fotefo kwacha pa wani handede iliyonse. Kalata yomwe bankiyi yatulutsa, ikuonetsa kuti izi zachitika pofuna kuthandizira kupezeka kwa ndalama za kunja
Female
komanso kuthana ndi mchitidwe ogulitsa ndalama za kunja pa mtengo okwera, poyerekeza ndi mtengo ogulitsira ndalamayi pa msika wa ndalama
komanso kuthana ndi mchitidwe ogulitsa ndalama za kunja pa mtengo okwera, poyerekeza ndi mtengo ogulitsira ndalamayi pa msika wa ndalama
Female
Anthu ochuluka ati izi zikhudza ntchito za malonda komanso zikuonetsera poyenera kusayendetsa bwino kwa chuma cha dziko
Anthu ochuluka ati izi zikhudza ntchito za malonda komanso zikuonetsera poyenera kusayendetsa bwino kwa chuma cha dziko
Female
Kampani yopanga mankhwala othandiza pa nthenda zosiyanasiyana ya Maranatha Natural Healing Ministries yati ipitiliza kulengezetsa malonda a mankhwala ake
Kampani yopanga mankhwala othandiza pa nthenda zosiyanasiyana ya Maranafa nachulo hiling’i minisitilezi yati ipitiliza kulengezetsa malonda a mankhwala ake
Female
mnyumba zowulutsira mawu ndi nyuzipepala zosiyanasiyana mdziko muno. Mkulu wa Maranatha Natural Healing Ministries, James Nkhutabasa
mnyumba zowulutsira mawu ndi nyuzipepala zosiyanasiyana mdziko muno. Mkulu wa Maranafa nachulo hiling’i minisitilezi, Jamusi Nkhutabasa
Female
wati kampani yawo yakwanilitsa ndondomeko zonse zomwe a bungwe lowona za mankhwala la Pharmacy and Regulatory Authority-PMRA
wati kampani yawo yakwanilitsa ndondomeko zonse zomwe a bungwe lowona za mankhwala la famase andi legyuletale ofolite –Piemualae
Female
ndi a bungwe la MACRA amafuna, mauthenga okhuza mankhwala otere asanatsindikizidwe. Pamenepa, iwo ati okondwa ndi kukulira-kulira kwa chikhulupiliro chomwe anthu akumakhala nacho mu ntchito zake
ndi a bungwe la MAKILA amafuna, mauthenga okhuza mankhwala otere asanatsindikizidwe. Pamenepa, iwo ati okondwa ndi kukulira-kulira kwa chikhulupiliro chomwe anthu akumakhala nacho mu ntchito zake
Female
Tikufuna tithokoze makasitomala athu potikhulupilira pa ntchito zathu ndipo tilonjeze kuti tipitilire kuwathandiza mokhulupirika ndi mowona mtima, atero a Nkhutabasa
Tikufuna tithokoze makasitomala athu potikhulupilira pa ntchito zathu ndipo tilonjeze kuti tipitilire kuwathandiza mokhulupirika ndi mowona mtima, atero a Nkhutabasa
Female
Atolankhani mdziko muno awapempha kuti ayike chidwi chawo pa kumvetsetsa nkhani za nyengo ndi kusintha kwa nyengo, ndi cholinga choti azifikira anthu ndi uthenga oyenera pa nkhanizi
Atolankhani mdziko muno awapempha kuti ayike chidwi chawo pa kumvetsetsa nkhani za nyengo ndi kusintha kwa nyengo, ndi cholinga choti azifikira anthu ndi uthenga oyenera pa nkhanizi
Female
Izitu ndi malingana ndi m'modzi wa achiwiri kwa mkulu wa nthambi yoona za nyengo ya DCCMS, Izitu ndi malingana ndi m'modzi wa achiwiri kwa mkulu wa nthambi yoona za nyengo
Izitu ndi malingana ndi m'modzi wa achiwiri kwa mkulu wa nthambi yoona za nyengo ya Disisiemuesi, Izitu ndi malingana ndi m'modzi wa achiwiri kwa mkulu wa nthambi yoona za nyengo
Female
ya DCCMS, a Charles Vanya omwe ati uthenga olondola pa momwe nyengo ikuyendera umathandizanso anthu kupanga ziganizo zoyenera mu nthawi yake
ya Disisiemuesi, a Tchalosi Vanya omwe ati uthenga olondola pa momwe nyengo ikuyendera umathandizanso anthu kupanga ziganizo zoyenera mu nthawi yake
Female
Ife ngati nthambi ya za nyengo timadalira atolankhani kuti anthu afikilidwe ndi ulosi wathu pa nyengo, atero a Vanya
Ife ngati nthambi ya za nyengo timadalira atolankhani kuti anthu afikilidwe ndi ulosi wathu pa nyengo, atero a Vanya
Female
Iwo ayankhula izi pa maphunziro okhuza za nyengo omwe bungwe lawo lakonzera atolankhani a za nyengo pansi pa bungwe la Network for Climate Journalists-NCJ
Iwo ayankhula izi pa maphunziro okhuza za nyengo omwe bungwe lawo lakonzera atolankhani a za nyengo pansi pa bungwe la netiweki fo kilaimeti jonalisitsi-Enisijei
Female
Ndipo m'mawu ake, wa pa mpando wa bungwe la NCJ, Dietrich Frederich wathokoza wathokoza DCCMS kaamba ka maphunzirowa
Ndipo m'mawu ake, wa pa mpando wa bungwe la Enisijei, Ditilichi Fulediliki wathokoza wathokoza Disisiemuesi kaamba ka maphunzirowa
Female
Ndipemphe atolankhani amnzanga kuti agwiritse ntchito maphunzirowa moyenelera chifukwa mwayi otere umasowa, atero a Frederick
Ndipemphe atolankhani amnzanga kuti agwiritse ntchito maphunzirowa moyenelera chifukwa mwayi otere umasowa, atero a Fulediliki
Female
Katswiri pa nkhani za mayimbidwe, Thomas Chibade wamwalira. Komabe, zambiri zokhuza nkhani ya chisoniyi sizinadziwike pakadali pano
Katswiri pa nkhani za mayimbidwe, Thomasi Chibade wamwalira. Komabe, zambiri zokhuza nkhani ya chisoniyi sizinadziwike pakadali pano
Female
Malemu Chibade anadziwika ndi nyimbo monga Awa ndiwo mau anga, Bulu wanding'amba nthiti komanso Our Love
Malemu Chibade anadziwika ndi nyimbo monga Awa ndiwo mau anga, Bulu wanding'amba nthiti komanso awa lavu
Female
A Maria Chiwaya komanso a Victoria Mvula apeza ndalama zokwana K250 thousand aliyense mu mpikisano wa Back to School omwe bank ya First Capital ikuchititsa
A Maria Chiwaya komanso a Vikitoliyaa Mvula apeza ndalama zokwana thu handiledi andi fifite saizande kwacha aliyense mu mpikisano wa Baki tu sukulu omwe banki ya Fesiti kapito ikuchititsa
Female
Iwo apeza ndalamazi m'maere achiwiri a pa mwezi omwe achitika lero. Mpikisanowu, malingana ndi banki-yi, ukufuna kuthandiza anthu ogwira ntchito m'boma kupeza ngongole zothandizira pa maphunziro a ana ndi abale awo
Iwo apeza ndalamazi m'maere achiwiri a pa mwezi omwe achitika lero. Mpikisanowu, malingana ndi banki-yi, ukufuna kuthandiza anthu ogwira ntchito m'boma kupeza ngongole zothandizira pa maphunziro a ana ndi abale awo
Female
Mkulu wa za malonda ku First Capital Bank, Pachalo Stanley Chiyora wawuza atolankhani kuti banki yawo ndi yokondwa ndi momwe mpikisanowu omwe ufike kumapeto mwezi wa mawa, ukuyendera
Mkulu wa za malonda ku fesiti kapito banki, Pachalo Sitanile Chiyora wawuza atolankhani kuti banki yawo ndi yokondwa ndi momwe mpikisanowu omwe ufike kumapeto mwezi wa mawa, ukuyendera
Female
Nthambi ya za nyengo ndi kusintha kwa nyengo yachenjeza kuti madera ambiri a dziko lino akumana ndi nyengo yotentha kwambiri kuyambira lero mpaka loweruka sabata ino
Nthambi ya za nyengo ndi kusintha kwa nyengo yachenjeza kuti madera ambiri a dziko lino akumana ndi nyengo yotentha kwambiri kuyambira lero mpaka loweruka sabata ino
Female
Malingana ndi nthambiyi, madera monga a ku chigwa cha mtsinje wa Shire kutentha mpaka madigiri 44 Celsius ndipo mphepete mwa nyanja kutentha 39 mpaka 40 digiri Celsius
Malingana ndi nthambiyi, madera monga a ku chigwa cha mtsinje wa Shire kutentha mpaka madigiri fotefolo sewoshazi ndipo mphepete mwa nyanja kutentha fete naini mpaka fote digiri sewoshazi
Female
Pamenepa, nthambiyi yalangiza anthu kumwa madzi pafupifupi ngakhale sakumva lunzu, kuvala zovala zomasuka bwino komanso apewe kumwa mowa, mwa zina
Pamenepa, nthambiyi yalangiza anthu kumwa madzi pafupifupi ngakhale sakumva lunzu, kuvala zovala zomasuka bwino komanso apewe kumwa mowa, mwa zina
Female
Oyimba wina, Elias Missi yemwe amadziwika ndi dzina loti Atoht Manje wamwalira. Malipoti akuti wamwalira usiku wapitawu koma gwero la imfa yake silinadziwike bwinobwino
Oyimba wina, Eliasi Missi yemwe amadziwika ndi dzina loti Atoti Manje wamwalira. Malipoti akuti wamwalira usiku wapitawu koma gwero la imfa yake silinadziwike bwinobwino
Female
Pakadali pano, anthu ayamba kale kukhuza maliro a oyimbayu yemwe amadziwika ndi nyimbo monga Kunong'a, Phone ya Bae, Woyo Woyo, Che Patuma komanso Huwa
Pakadali pano, anthu ayamba kale kukhuza maliro a oyimbayu yemwe amadziwika ndi nyimbo monga Kunong'a, foni ya Bae, Woyo Woyo, Che Patuma komanso Huwa
Female
Nduna ya zofalitsa nkhani, a Moses Kunkuyu ati mtsogoleri wa dziko lino, Lazarus Chakwera wakumana ndi anthu osiyanasiyana
Nduna ya zofalitsa nkhani, a Mozesi Kunkuyu ati mtsogoleri wa dziko lino, Lazalasi Chakwera wakumana ndi anthu osiyanasiyana
Female
omwe ali okonzeka kuthandiza dziko lino mu njira zosiyanasiyana, pa ulendo wake wa posachedwapa wa ku msonkhano wa mgwirizano wa mayiko onse wa UNGA
omwe ali okonzeka kuthandiza dziko lino mu njira zosiyanasiyana, pa ulendo wake wa posachedwapa wa ku msonkhano wa mgwirizano wa mayiko onse wa UNGA
Female
Iwo anena izi pa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Lilongwe komwenso akuti ulendowo uthandiza dziko lino kuthana ndi mavuto ena omwe likukumana nalo
Iwo anena izi pa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Lilongwe komwenso akuti ulendowo uthandiza dziko lino kuthana ndi mavuto ena omwe likukumana nalo
Female
Ku m'mawaku, anamwino omwe anamaliza maphunziro awo a degree msukulu za ukachenjede koma sanalembedwe ntchito, achita zionetsero mu mzinda wa Blantyre pofuna kukakamiza boma kuti liwalembe ntchito
Ku m'mawaku, anamwino omwe anamaliza maphunziro awo a digili msukulu za ukachenjede koma sanalembedwe ntchito, achita zionetsero mu mzinda wa Bulantaya pofuna kukakamiza boma kuti liwalembe ntchito
Female
Tayankhula ndi wa pa mpando wa gulu la anamwinowa, Frank Kamwendo yemwe watiwuza kuti ena mwa iwo akhala pakhomo kwa zaka zopitilira zinayi
Tayankhula ndi wa pa mpando wa gulu la anamwinowa, Fulanki Kamwendo yemwe watiwuza kuti ena mwa iwo akhala pakhomo kwa zaka zopitilira zinayi
Female
kuchokera pomwe anamaliza maphunziro awo pa unamwinowo, ndipo ena atopa kugwira ntchito mwa ganyu chabe yomwenso akuti malipiro ake amakhala ochepa
kuchokera pomwe anamaliza maphunziro awo pa unamwinowo, ndipo ena atopa kugwira ntchito mwa ganyu chabe yomwenso akuti malipiro ake amakhala ochepa
Female
Anamwinowa asiya kalata ya madandawulo awo ku ofesi za khonsolo ya boma la Blantyre kuti itumizidwe kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera
Anamwinowa asiya kalata ya madandawulo awo ku ofesi za khonsolo ya boma la Bulantaya kuti itumizidwe kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dokota. Lazalasi Chakwera
Female