audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
apolisi atamumanga sabata zapitazo pambuyo polandira dandawulo kuchokera kwa olakwilidwa mu nkhaniyi | apolisi atamumanga sabata zapitazo pambuyo polandira dandawulo kuchokera kwa olakwilidwa mu nkhaniyi | Female | |
Ofalitsa nkhani za apolisi ku Limbe, Aubrey Singanyama wati bwaloli linamva kudzera mwa yemwe amayimira boma pa mlanduwu, Grace Kanjiwa | Ofalitsa nkhani za apolisi ku Limbe, Obule Singanyama wati bwaloli linamva kudzera mwa yemwe amayimira boma pa mlanduwu, Gilesi Kanjiwa | Female | |
kuti Majawa anagawa kanemayu mmagulupu a pa WhatsApp ku kachisi komanso ku sukulu. Komatu poonekera m'bwalo la milandu, opalamulayu anawukana mlanduwu | kuti Majawa anagawa kanemayu mmagulupu a pa watsapup ku kachisi komanso ku sukulu. Komatu poonekera m'bwalo la milandu, opalamulayu anawukana mlanduwu | Female | |
koma mbali ya boma inabweretsa mboni ziwiri kutsimikizira za nkhaniyi zomwe zinachititsa kuti oweluza Sajida Maiden kupeleka chilango chotere | koma mbali ya boma inabweretsa mboni ziwiri kutsimikizira za nkhaniyi zomwe zinachititsa kuti oweluza Sajida Maideni kupeleka chilango chotere | Female | |
Olakwilidwa pa nkhaniyi alandira ndalama zokwana K190 thousand. Ku Mangochi Malipoti akuti mzika za m'mayiko ena zopitilira 50 | Olakwilidwa pa nkhaniyi alandira ndalama zokwana wanu handiledi andi nainte sauzande kwacha. Ku Mangochi Malipoti akuti mzika za m'mayiko ena zopitilira fifite | Female | |
zomwe zimakhala ku m'bomali zabwelera ku msasa wa Dzaleka. Apolisi komanso ogwira ku nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka | zomwe zimakhala ku m'bomali zabwelera ku msasa wa Dzaleka. Apolisi komanso ogwira ku nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka | Female | |
ya Immigration anagwira anthuwa usiku wapitawu ndipo anakawasunga pa bwalo la zamasewero la Mangochi, asanawatumize ku msasawu lero | ya Imigileshoni anagwira anthuwa usiku wapitawu ndipo anakawasunga pa bwalo la zamasewero la Mangochi, asanawatumize ku msasawu lero | Female | |
Ntchitoyi ikutichitika dziko lino, ndipo anthuwa akukakamizidwa kubwelera ku msasawu, nthawi yomwe boma linapereka kuti abwelere mwa okha, itatha | Ntchitoyi ikutichitika dziko lino, ndipo anthuwa akukakamizidwa kubwelera ku msasawu, nthawi yomwe boma linapereka kuti abwelere mwa okha, itatha | Female | |
Apolisi ku Blantyre akusamusa anthu othawa kwawo omwe akukhala kunja kwa msasa wa Dzaleka. Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi mchigawo cha kum'mwera ku madzulo | Apolisi ku Bulantaya akusamusa anthu othawa kwawo omwe akukhala kunja kwa msasa wa Dzaleka. Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi mchigawo cha kum'mwera ku madzulo | Female | |
Beatrice Mikuwa watsimikiza za izi koma watiwuza kuti tifunse tsatanetsatane wa nkhaniyi mneneri wa apolisi mdziko muno, a Peter Kalaya | Bitilisi Mikuwa watsimikiza za izi koma watiwuza kuti tifunse tsatanetsatane wa nkhaniyi mneneri wa apolisi mdziko muno, a Pita Kalaya | Female | |
Koma munthu wina yemwe waona izi zikuchitika koma wati tisamutchule dzina watiwuza kuti ku dera la Kanjedza apolisi akumalowa mnyumba ndikutenga anthu onse kukawakweza galimoto zawo | Koma munthu wina yemwe waona izi zikuchitika koma wati tisamutchule dzina watiwuza kuti ku dera la Kanjedza apolisi akumalowa mnyumba ndikutenga anthu onse kukawakweza galimoto zawo | Female | |
Ndaona mayi wina akusiyisidwa kumwa tea ndikumuwuza kuti akakwere galimoto, azipita, watero munthuyu | Ndaona mayi wina akusiyisidwa kumwa teyi ndikumuwuza kuti akakwere galimoto, azipita, watero munthuyu | Female | |
Mulandu omwe anthu ena awiri akufuna bwalo la milandu ligamule kuti malamulo oletsa mchitidwe wa mathanyula akuphwanya malamulo akulu a dziko lino upitilira pa 5 ndi pa 6 June chaka chino | Mulandu omwe anthu ena awiri akufuna bwalo la milandu ligamule kuti malamulo oletsa mchitidwe wa mathanyula akuphwanya malamulo akulu a dziko lino upitilira pa faifi ndi pa sikisi Juni chaka chino | Female | |
koma zomwe MCP ikuchita ziwathandiza kudziwilatu anthu oyenela, atelo a Thindwa. Bank ya first capital FCB | koma zomwe emusipi ikuchita ziwathandiza kudziwilatu anthu oyenela, atelo a Thindwa. Banki ya fesiti kapito efusibi | Female | |
Mzika ya dziko la Netherlands, Jan Willem Akstar komanso mai Jana Gonani aku Mangochi ndi omwe anapeleka pempholi ku bwalo la milandu | Mzika ya dziko la Nevelanzis, Jani Wilemu Aksita komanso mai Jana Gonani aku Mangochi ndi omwe anapeleka pempholi ku bwalo la milandu | Female | |
Nkhaniyi yakwiyitsa mabungwe akuluakulu a zipembedzo m'dziko muno omwe akuti maukwati a amayi kapena amuna okha-okha ndi uchimo pa maso pa Mulungu | Nkhaniyi yakwiyitsa mabungwe akuluakulu a zipembedzo m'dziko muno omwe akuti maukwati a amayi kapena amuna okha-okha ndi uchimo pa maso pa Mulungu | Female | |
Oweruza milandu a bwalo lalikulu atatu omwe ndi aJoseph Chigona, aVikochi Chima komanso a Chimbizgani Kacheche | Oweruza milandu a bwalo lalikulu atatu omwe ndi a jozefe Chigona, a Vikochi Chima komanso a Chimbizani Kacheche | Female | |
amayenera kupitilira kumva mulanduwu lero, Lachiwiri, koma zasintha. Komabe ngakhale izi zili chomwechi, mabungwe ena omenyera ufulu wa ana akufuna kuti a Akstar | amayenera kupitilira kumva mulanduwu lero, Lachiwiri, koma zasintha. Komabe ngakhale izi zili chomwechi, mabungwe ena omenyera ufulu wa ana akufuna kuti a Akisita | Female | |
ayimbidwebe milandu yophwanya ufulu wa ana potengera zomwe anachita. AMemory Chisenga ndi mmodzi mwa omenyera maufulu a anawa ndipo akugwira ntchito limodzi ndi mabungwewa | ayimbidwebe milandu yophwanya ufulu wa ana potengera zomwe anachita. A Memole Chisenga ndi mmodzi mwa omenyera maufulu a anawa ndipo akugwira ntchito limodzi ndi mabungwewa | Female | |
Iwo akuti chilungamo chikuyenera kuyenda ngati madzi posatengera kuti a Akstar ali ndi mphanvu komanso chuma chochuluka bwanji | Iwo akuti chilungamo chikuyenera kuyenda ngati madzi posatengera kuti a Akisita ali ndi mphanvu komanso chuma chochuluka bwanji | Female | |
Iwo awuza olemba nkhani ku Blantyre kuti ndi zokhumudwitsa kuti mlanduwu ukuyenda pang'ono-pang'ono koma ati ali ndi chikhulupiliro ndi mabwalo a milandu kuti zonse ziyenda bwino | Iwo awuza olemba nkhani ku Bulantaya kuti ndi zokhumudwitsa kuti mlanduwu ukuyenda pang'ono-pang'ono koma ati ali ndi chikhulupiliro ndi mabwalo a milandu kuti zonse ziyenda bwino. | Female | |
Akstar akuwaganizira kuti anapalamula mlanduwu mchaka cha 2020. Mabungwe komanso anthu osiyanasiyana awapempha kuti ayambe kuyika chidwi | Akisita akuwaganizira kuti anapalamula mlanduwu mchaka cha twente twente. Mabungwe komanso anthu osiyanasiyana awapempha kuti ayambe kuyika chidwi | Female | |
ku nkhani za masewero ngati imodzi mwa njira yothanirana ndi mchitidwe opalamula milandu komanso nkhanza zochitirana pakati pa amuna ndi akazi | ku nkhani za masewero ngati imodzi mwa njira yothanirana ndi mchitidwe opalamula milandu komanso nkhanza zochitirana pakati pa amuna ndi akazi | Female | |
Pempholi laperekedwa ndi mkulu wina ochita malonda wa m'boma la Thyolo, Patrick Maningi pa masewero a mpira wa miyendo | Pempholi laperekedwa ndi mkulu wina ochita malonda wa m'boma la Thyolo, Patiliki Maningi pa masewero a mpira wa miyendo | Female | |
a mu ndime yotsiriza ya chikho cha TryJesus chomwe chinali cha ndalama zokwana K200 thousand zomwe anapeleka anapeleka iye | a mu ndime yotsiriza ya chikho cha Tyhilaijizasi chomwe chinali cha ndalama zokwana thu handiledi sauzande kwacha zomwe anapeleka anapeleka iye | Female | |
Chikhochi chimakhuza matimu a mpira wa miyendo a m'boma la Thyolo. Pa masewero a ndime yotsirizawa omwe achitika kumathero a sabata yathayi pa bwalo la za masewero la Molele | Chikhochi chimakhuza matimu a mpira wa miyendo a m'boma la Thyolo. Pa masewero a ndime yotsirizawa omwe achitika kumathero a sabata yathayi pa bwalo la za masewero la Molele | Female | |
timu ya Masambanjati Select yakhala akatswiri pomwe yagonjetsa timu ya Chimzama FC. Mwa zina, akatswiriwa apeza ndalama zokwana K100 thousand | timu ya Masambanjati selekiti yakhala akatswiri pomwe yagonjetsa timu ya Chimzama efusi. Mwa zina, akatswiriwa apeza ndalama zokwana wani handiiledi sauzande kwacha | Female | |
pamene owatsatira awo apeza ndalama zokwana K60 thousand ngati mphoto. Pamenepa, Maningi wati | pamene owatsatira awo apeza ndalama zokwana sikisite sauzande kwacha ngati mphoto. Pamenepa, Maningi wati | Female | |
ndi okondwa kuti mpikisanowu wayenda bwino potengera kuti wathandiza kupeleka chochita kwa achinyamata omwe ndi tsogolo la dziko lino | ndi okondwa kuti mpikisanowu wayenda bwino potengera kuti wathandiza kupeleka chochita kwa achinyamata omwe ndi tsogolo la dziko lino | Female | |
Pomwe mtsutso pa nkhani yoti anthu othawa kwawo omwe akukhala kunja kwa msasa wa Dzaleka abwelere ku msasawu ukupitilira | Pomwe mtsutso pa nkhani yoti anthu othawa kwawo omwe akukhala kunja kwa msasa wa Dzaleka abwelere ku msasawu ukupitilira | Female | |
makomiti Oona za chitetezo, malonda komanso ubale wa dziko lino ndi mayiko ena a ku nyumba ya malamulo ayikira kumbuyo boma pa ganizoli | makomiti Oona za chitetezo, malonda komanso ubale wa dziko lino ndi mayiko ena a ku nyumba ya malamulo ayikira kumbuyo boma pa ganizoli | Female | |
Makomitiwa ati zomwe anthu othawa kwawowa amachita, mwa Zina, ntchito za malonda zimaonetsa ngati malamulo a dziko lino ndi opanda pake komanso anthuwa amabweretsa chisokonezo | Makomitiwa ati zomwe anthu othawa kwawowa amachita, mwa Zina, ntchito za malonda zimaonetsa ngati malamulo a dziko lino ndi opanda pake komanso anthuwa amabweretsa chisokonezo | Female | |
Boma kudzera mu unduna wa za chitetezo Cha m'dziko wakhala ukuti anthuwa amayenera ku msasa wa Dzaleka basi | Boma kudzera mu unduna wa za chitetezo Cha m'dziko wakhala ukuti anthuwa amayenera ku msasa wa Dzaleka basi | Female | |
pokhapokha apeze kalata zoyenelera zochitira bizinesi kapena kukhala malo ena, mdziko muno. Komabe, mabungwe komanso anthu ena akutsutsana ndi izi ponena kuti pali kuphwanya kwa ufulu wa anthuwa | pokhapokha apeze kalata zoyenelera zochitira bizinesi kapena kukhala malo ena, mdziko muno. Komabe, mabungwe komanso anthu ena akutsutsana ndi izi ponena kuti pali kuphwanya kwa ufulu wa anthuwa | Female | |
Apolisi ku Balaka atsimikiza kuti bambo wa zaka 20. Apolisi ku Balaka atsimikiza kuti bambo wa zaka 20, Madalitso Banda | Apolisi ku Balaka atsimikiza kuti bambo wa zaka twente. Apolisi ku Balaka atsimikiza kuti bambo wa zaka twente, Madalitso Banda | Female | |
wazipha pozimangilira ku denga la nyumba atakangana ndi mkazi wake, pa nkhani za m'banja. Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi ku Balaka, Mphatso Munthali | wazipha pozimangilira ku denga la nyumba atakangana ndi mkazi wake, pa nkhani za m'banja. Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi ku Balaka, Mphatso Munthali | Female | |
wati Banda ndi mkazi wake anakangana mpaka kumenyana loweluka sabata yatha, malemuyu asanazimangilire | wati Banda ndi mkazi wake anakangana mpaka kumenyana loweluka sabata yatha, malemuyu asanazimangilire | Female | |
M'modzi wa alakatuli mdziko muno, Raphael Sitima wati atulutsa ndakatulo yatsopano. Ndakatuloyi yomwe mutu wake akuti Okhwelhana Womalha, ituluka nthawi ya 7 koloko madzulo | M'modzi wa alakatuli mdziko muno, Rafaelo Sitima wati atulutsa ndakatulo yatsopano. Ndakatuloyi yomwe mutu wake akuti Okhwelana Womala, ituluka nthawi ya seveni koloko madzulo | Female | |
ndipo ili muziyankhulo za Chingerezi, Chichewa komanso Chilomwe. Mkuluyu adalakatulopo ndakatulo zina zodziwika bwino monga Chala Changa, Kwathu, Pemphero | ndipo ili muziyankhulo za Chingerezi, Chichewa komanso Chilomwe. Mkuluyu adalakatulopo ndakatulo zina zodziwika bwino monga Chala Changa, Kwathu, Pemphero | Female | |
Ulendo Wa Dorika, Kuteteza ndi Kotsalako. A Atupele Muluzi sakunenabe mwatchutchutchu | Ulendo Wa Dorika, Kuteteza ndi Kotsalako. A Atupele Muluzi sakunenabe mwatchutchutchu | Female | |
Pomwe anthu amayembekezera kuti amva yankho pa pempho lomwe anapeleka kuti ayime, a Muluzi ayankhula mozungulirazungulira koma anthu ena akuti, uku ndi kuvomera pempholi mwachikulu | Pomwe anthu amayembekezera kuti amva yankho pa pempho lomwe anapeleka kuti ayime, a Muluzi ayankhula mozungulirazungulira koma anthu ena akuti, uku ndi kuvomera pempholi mwachikulu | Female | |
Amalawi, ndizayima nanu nthawi zonse maka pa nthawi ya mavuto, atero a Muluzi. A Muluzi ati chipani chawo chipita ku msonkhano wake wa ukulu posachedwapa | Amalawi, ndizayima nanu nthawi zonse maka pa nthawi ya mavuto, atero a Muluzi. A Muluzi ati chipani chawo chipita ku msonkhano wake wa ukulu posachedwapa | Female | |
kukasankha adindo ndipo apempha anthu Maka achinyamata kuti aonetse chidwi chozapikisana nawo mmaudindo osiyanasiyana Iwo apemphanso anthu ena omwe anali mamembala a UDF kuti abwelere | kukasankha adindo ndipo apempha anthu Maka achinyamata kuti aonetse chidwi chozapikisana nawo mmaudindo osiyanasiyana Iwo apemphanso anthu ena omwe anali mamembala a yudiefu kuti abwelere | Female | |
pofuna kukonzera limodzi chipanichi. Poyankhula pa msonkhanowu, yemwe anakhalako mtsogoleri wa UDF, Atupele Muluzi | pofuna kukonzera limodzi chipanichi. Poyankhula pa msonkhanowu, yemwe anakhalako mtsogoleri wa yudiefu, Atupele Muluzi | Female | |
wapempha adindo kuti athandize anthu a chigawo cha ku m'mwera omwe anataya ziphatso zawo za umzika ku namondwe wa Freddy, ndi ziphatsozi mwa msanga ponena kuti zinthu zambiri masiku ano zikumafunikira ziphaso | wapempha adindo kuti athandize anthu a chigawo cha ku m'mwera omwe anataya ziphatso zawo za umzika ku namondwe wa Fulede, ndi ziphatsozi mwa msanga ponena kuti zinthu zambiri masiku ano zikumafunikira ziphaso | Female | |
A Muluzi, anayamba ndi kupempha anthu kuti ayimire pokumbukira miyoyo ya anthu omwe anamwalira ndi namondweyu | A Muluzi, anayamba ndi kupempha anthu kuti ayimire pokumbukira miyoyo ya anthu omwe anamwalira ndi namondweyu | Female | |
Phungu wa ku nyumba ya malamulo oimira dera la Ndirande Malabada, Ishmael Mkumba wadandawula kaamba kakukula kwa ulova komanso umphawi mdziko muno | Phungu wa ku nyumba ya malamulo oimira dera la Ndirande Malabada, Ishumaeli Mkumba wadandawula kaamba kakukula kwa ulova komanso umphawi mdziko muno | Female | |
A Mkumba ati anthu akulimbikira ntchito, koma zinthu zikuvutabe pakati pawo. Anthu ayembekezere kuti zinthu zivutabe | A Mkumba ati anthu akulimbikira ntchito, koma zinthu zikuvutabe pakati pawo. Anthu ayembekezere kuti zinthu zivutabe | Female | |
ndipo tikuyenera kulimbika zedi kuti zizafike pithiniratu, atero a Mkumba. Pamenepa, iwo ati pali njira zingapo zomwe anthu a mdera lawo akutsata pofuna kuthana ndi mavutowa | ndipo tikuyenera kulimbika zedi kuti zizafike pithiniratu, atero a Mkumba. Pamenepa, iwo ati pali njira zingapo zomwe anthu a mdera lawo akutsata pofuna kuthana ndi mavutowa | Female | |
ndipo njirazi zili pansi pa kampani ya Ndirande Trust. Pansi pa kampani ya Ndirande Trust, Pali kampani yopanga Madzi komanso SACCO | ndipo njirazi zili pansi pa kampani ya Ndirande Thilasiti. Pansi pa kampani ya Ndirande Thilasiti, Pali kampani yopanga Madzi komanso sako | Female | |
Ndinamva kuti anthu ena anabwera ku nyumba kwanu masiku apitawo kuzapereka pempho, ndikhulupilira yankho lake muli nalo | Ndinamva kuti anthu ena anabwera ku nyumba kwanu masiku apitawo kuzapereka pempho, ndikhulupilira yankho lake muli nalo | Female | |
Awatu ndi mawu a mfumu Somanje Makata ya ku Ndirande ndipo ayankhula pomwe amalandira anthu pa msonkhano omwe UDF ikuchititsa pa Nyambadwe ground | Awatu ndi mawu a mfumu Somanje Makata ya ku Ndirande ndipo ayankhula pomwe amalandira anthu pa msonkhano omwe yudiefu ikuchititsa pa Nyambadwe gilaundi | Female | |
Mawu awo akudza kutsatira ulendo wa ndalama omwe amayenda mamembala ena a UDF kulunjika ku nyumba ya a Muluzi kukapempha kuti ayimirenso UDF pa chisankho cha mtsogoleri mchaka cha 2025 | Mawu awo akudza kutsatira ulendo wa ndalama omwe amayenda mamembala ena a yudiefu kulunjika ku nyumba ya a Muluzi kukapempha kuti ayimirenso yudiefu pa chisankho cha mtsogoleri mchaka cha twene twente faifi | Female | |
Malingana ndi a Somanje Makata, chiyembekezo Cha anthu ndi choti adziwa tsogolo lenileni la a Muluzi. Ogwirizira udindo wa mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front-UDF | Malingana ndi a Somanje Makata, chiyembekezo Cha anthu ndi choti adziwa tsogolo lenileni la a Muluzi. Ogwirizira udindo wa mtsogoleri wa chipani cha yunaitedi demokilatiki fulanti- Yudiefu | Female | |
Lilian Patel sapezeka nawo pa msonkhano wa ndale omwe chipanichi chikuchititsa pa bwalo la za masewero la Nyambadwe ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre | Liliyani Patel sapezeka nawo pa msonkhano wa ndale omwe chipanichi chikuchititsa pa bwalo la za masewero la Nyambadwe ku Ndirande mu mzinda wa Bulantaya | Female | |
Dzulo, mneneri wa chipanichi, a Yusuf Mwawa anatiwuza kuti a Patel apezeka, koma malingana ndi zomwe oyendetsa mwambowo anena | Dzulo, mneneri wa chipanichi, a Yusufu Mwawa anatiwuza kuti a Patel apezeka, koma malingana ndi zomwe oyendetsa mwambowo anena | Female | |
mtsogoleriyu ali ku Scotland komwe akugwira ntchito Zina ngati phungu wa ku nyumba malamulo. Pakadali pano, msonkhanowu wayamba | mtsogoleriyu ali ku Sikotilandi komwe akugwira ntchito Zina ngati phungu wa ku nyumba malamulo. Pakadali pano, msonkhanowu wayamba | Female | |
ndipo yemwe anali mtsogoleri wake m'mbuyomu, a Atupele Muluzi komanso anthu ena omwe ndi akuluakulu aku UDF, afika | ndipo yemwe anali mtsogoleri wake m'mbuyomu, a Atupele Muluzi komanso anthu ena omwe ndi akuluakulu aku Yudiefu, afika | Female | |
Chipani cha United Democratic Front-UDF lero chichititsa msonkhano wa ndale pa bwalo la za masewero la Nyambadwe ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre | Chipani cha Yunaitedi demokilatiki fulanti-Yudiefu lero chichititsa msonkhano wa ndale pa bwalo la za masewero la Nyambadwe ku Ndirande mu mzinda wa Bulantaya | Female | |
komwe malingana ndi mneneri wake, a Yusuf Mwawa, anthu ayembekezere kumva mfundo zokuza dziko lino pa chuma komanso utsogoleri okomera onse | komwe malingana ndi mneneri wake, a Yusufu Mwawa, anthu ayembekezere kumva mfundo zokuza dziko lino pa chuma komanso utsogoleri okomera onse | Female | |
A Mwawa, poyankhula nafe dzulo, anati mlendo olemekezeka pa msonkhanowu akhala mtsogoleri wa chipanichi, a Lilian Patel | A Mwawa, poyankhula nafe dzulo, anati mlendo olemekezeka pa msonkhanowu akhala mtsogoleri wa chipanichi, a Liliyani Patel | Female | |
Iwo atinso yemwe anali mtsogoleri wake m'mbuyomu, a Atupele Muluzi apezeka ndipo ayankhula mfundo zomanga chipani, mwa Zina | Iwo atinso yemwe anali mtsogoleri wake m'mbuyomu, a Atupele Muluzi apezeka ndipo ayankhula mfundo zomanga chipani, mwa Zina | Female | |
Pamenepa, mneneri wa UDF-yu wamema anthu kuti akhamukire pa bwaloli ndipo kuti msonkhanowu uyamba 2 koloko masana | Pamenepa, mneneri wa yudiefu-yu wamema anthu kuti akhamukire pa bwaloli ndipo kuti msonkhanowu uyamba thu koloko masana | Female | |
Ngakhale vuto la kusowa kwa mafuta a galimoto likuoneka kuti lachepa, anthu ena oyendetsa minibus Maka ku Blantyre sanasitsebe mitengo yomwe amalipilitsa mitengo ya anthu a pa ulendo | Ngakhale vuto la kusowa kwa mafuta a galimoto likuoneka kuti lachepa, anthu ena oyendetsa minibasi Maka ku Bulantaya sanasitsebe mitengo yomwe amalipilitsa mitengo ya anthu a pa ulendo | Female | |
Mitengoyi inakwera sabata zapitazo, kaamba koti mafuta amasowa, ndipo eni galimoto amayenda maulendo atalitali komanso kukhala pa mnzere kwa nthawi yayitali pofuna mafutawa | Mitengoyi inakwera sabata zapitazo, kaamba koti mafuta amasowa, ndipo eni galimoto amayenda maulendo atalitali komanso kukhala pa mnzere kwa nthawi yayitali pofuna mafutawa | Female | |
Pomwe mafutawa ayamba kupezeka tsopano, anthu anali ndi chiyembekezo kuti azilipira ndalama zokwana K400 pochoka mu Limbe kukafika ku Blantyre | Pomwe mafutawa ayamba kupezeka tsopano, anthu anali ndi chiyembekezo kuti azilipira ndalama zokwana fohandede kwacha pochoka mu Limbe kukafika ku Bulantaya | Female | |
koma kwa sabata tsopano, anthu akulipirabe mtengo wa tsopano wa k 500a. Ichi ndi chitsanzo chabe Cha Madera angapo omwe mitengo sinabwelere mchimake | koma kwa sabata tsopano, anthu akulipirabe mtengo wa tsopano wa faifi handede kwacha. Ichi ndi chitsanzo chabe Cha Madera angapo omwe mitengo sinabwelere mchimake | Female | |
Mmbuyomu, bungwe la eni minibus mdziko muno la Minibus Owners Association of Malawi MOAM anatsimikizira wailesi ina kuti mitengoyi ibwelera mchimake mafuta akayamba kupezeka bwinobwino | Mmbuyomu, bungwe la eni minibasi mdziko muno la Minibasi Onazi asosieshoni ofu Malawi MOWAMU anatsimikizira wailesi ina kuti mitengoyi ibwelera mchimake mafuta akayamba kupezeka bwinobwino | Female | |
Mphunzitsi wa timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya Flames, Patrick mabedi | Mphunzitsi wa timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya Fulemuzi, Patiliki mabedi | Female | |
watulutsa mndandanda wa anyamata omwe ayambe kuchita zokonzekera za masewero a ndime yozigulira malo mu mpikisano wa matimu a mu Africa wa AFCON wa chaka chino | watulutsa mndandanda wa anyamata omwe ayambe kuchita zokonzekera za masewero a ndime yozigulira malo mu mpikisano wa matimu a mu Afulika wa Afukoni wa chaka chino | Female | |
Uwu ndiwo mndandanda wa osewera omwe akuyenera kuyamba nawo zokonzekerazi, lolemba likubwerali Otchinga pa golo, Osewera kumbuyo, Osewera pakati komanso Osewera kutsogolo | Uwu ndiwo mndandanda wa osewera omwe akuyenera kuyamba nawo zokonzekerazi, lolemba likubwerali Otchinga pa golo, Osewera kumbuyo, Osewera pakati komanso Osewera kutsogolo | Female | |
Zotsatira za kuyeza koyamba kwa thupi la mtolankhani wina, Nomsa Taulo yemwe anamwalira mwazidzidzi ku Lilongwe zasonyeza kuti imfa inali kaamba ka poison | Zotsatira za kuyeza koyamba kwa thupi la mtolankhani wina, Nomusa Taulo yemwe anamwalira mwazidzidzi ku Lilongwe zasonyeza kuti imfa inali kaamba ka poizoni | Female | |
Nomsa, yemwe amagwira ntchito yake ku nthambi ya zofalitsa nkhani ya bungwe la United Nations Development Programme (UNDP) mdziko la South Sudan | Nomusa, yemwe amagwira ntchito yake ku nthambi ya zofalitsa nkhani ya bungwe la Yunaitedi neshonzi divelopumenti pulogilamu (yuenidipi) mdziko la Saufi Sudani | Female | |
anamwalira pa 6 May chaka chino, atangofika m'dziko muno momwe anabwera ngati ku tchuthi. Ndirande FM yagwira mawu a tsamba lina mu nyuzipepala ya The Nation Publications Limited | anamwalira pa sikisi meyi chaka chino, atangofika m'dziko muno momwe anabwera ngati ku tchuthi. Ndirande efuemu yagwira mawu a tsamba lina mu nyuzipepala ya ve neshonzi pabulikeshonzi limitedi | Female | |
omwe amalume ake a Nomsa, a Mylord Jere akuti ndi odabwa komanso okhumudwa ndi malipoti oti mdzukulu wawo anamwalira ndi poison | omwe amalume ake a Nomusa, a Mailodi Jere akuti ndi odabwa komanso okhumudwa ndi malipoti oti mdzukulu wawo anamwalira ndi poizoni | Female | |
Tinamva za imfayi kudzera pa msamba a mchezo, nditapita ku nyumba kwake, ndinapeza anthu achilendo zomwe zinadzetsa mafunso. Ndinali osweka mtima, atero a Jere powuza nyuzipepalayi | Tinamva za imfayi kudzera pa msamba a mchezo, nditapita ku nyumba kwake, ndinapeza anthu achilendo zomwe zinadzetsa mafunso. Ndinali osweka mtima, atero a Jere powuza nyuzipepalayi | Female | |
Pakadali pano, anthu komanso magulu osiyanasiyana ayamba kale kufunsa adindo kuti afufuze mozama za nkhaniyi | Pakadali pano, anthu komanso magulu osiyanasiyana ayamba kale kufunsa adindo kuti afufuze mozama za nkhaniyi | Female | |
Apolisi amanga bambo wa zaka 39, Geoffrey Chavula pomuganizira kuti wakhala akuba galimoto za anthu omwe amamulemba ntchito ngati dalaivala wa matola | Apolisi amanga bambo wa zaka fetenaini, Jofule Chavula pomuganizira kuti wakhala akuba galimoto za anthu omwe amamulemba ntchito ngati dalaivala wa matola | Female | |
Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi mchigawo cha ku mpoto, Sub-Inspector Augustus Nkhwazi wati mkuluyu wamangidwa lachiwiri sabata ino | Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi mchigawo cha ku mpoto, sabu insipekita ogasitasi Nkhwazi wati mkuluyu wamangidwa lachiwiri sabata ino | Female | |
kutsatira kafukufuku yemwe amachitika malipoti okhuza kubedwa kwa galimoto atachuluka. Tikamaliza kafukuku, Chavula atsegulilidwa milandu yokhuza umbanda, atero a Nkhwazi | kutsatira kafukufuku yemwe amachitika malipoti okhuza kubedwa kwa galimoto atachuluka. Tikamaliza kafukuku, Chavula atsegulilidwa milandu yokhuza umbanda, atero a Nkhwazi | Female | |
Bungwe la CDEDI lati kuyambira lolemba sabata ya m'mawa liyamba kuchita m'bindikiro ku ofesi ya mlangizi wa boma pa nkhani za malamulo, Thabo Chakaka Nyirenda | Bungwe la Sidedi lati kuyambira lolemba sabata ya m'mawa liyamba kuchita m'bindikiro ku ofesi ya mlangizi wa boma pa nkhani za malamulo, Thabo Chakaka Nyirenda | Female | |
pofuna kumukakamiza kuti afotokozere momwe ntchito yobwezeretsa ndalama zokwana K750 million za ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya chaka chatha | pofuna kumukakamiza kuti afotokozere momwe ntchito yobwezeretsa ndalama zokwana thu handede andi sevente faifi miliyoni za ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya chaka chatha | Female | |
zomwe zinasowa ku kampami ina yogulitsa nyama ku UK, ikuyendera. M'bindikirowu umayenera kuyamba sabata yatha koma ofesiyi kudzera kwa bwanamkubwa wa boma la Lilongwe | zomwe zinasowa ku kampami ina yogulitsa nyama ku yukei, ikuyendera. M'bindikirowu umayenera kuyamba sabata yatha koma ofesiyi kudzera kwa bwanamkubwa wa boma la Lilongwe | Female | |
inapempha kuti pakhake zokambirana pakati pambali ziwirizi, zomwe malingana ndi mkulu wa CDEDI, Sylvester Namiwa, zokambiranazi sizinayitanitsidwe | inapempha kuti pakhake zokambirana pakati pambali ziwirizi, zomwe malingana ndi mkulu wa sidedi, Silivesita Namiwa, zokambiranazi sizinayitanitsidwe | Female | |
Poyankhula pa msonkhano wa atolankhani lero ku Lilongwe, a Namiwa ati adziwitsa kale ofesi ya bwanamkubwa wa boma la Lilongwe za chizokonzero za m'bindikiro cha tsopanochi | Poyankhula pa msonkhano wa atolankhani lero ku Lilongwe, a Namiwa ati adziwitsa kale ofesi ya bwanamkubwa wa boma la Lilongwe za chizokonzero za m'bindikiro cha tsopanochi | Female | |
A Chakaka-Nyirenda akhala akuti ofesi yawo ikuchilimika kuti ndalamazi zibwezedwe kuchokera pomwe zinadziwika kuti boma lapusisidwa, pa malonda ogula zipangizozo, mchaka chatha | A Chakaka-Nyirenda akhala akuti ofesi yawo ikuchilimika kuti ndalamazi zibwezedwe kuchokera pomwe zinadziwika kuti boma lapusisidwa, pa malonda ogula zipangizozo, mchaka chatha | Female | |
Bungwe loona za ufulu wa anthu la Malawi Human Rights Commission-MHRC lati lifufuza za malipoti a nkhanza zomwe akuti anthu othawa kwawo | Bungwe loona za ufulu wa anthu la Malawi Hyumani laitsi komishoni-emuetchialasi lati lifufuza za malipoti a nkhanza zomwe akuti anthu othawa kwawo | Female | |
omwe akukhala kunja kwa msasa wa Dzaleka achitilidwa ndi apolisi komanso a ku nthambi ya zolowa ndi zotuluka mdziko muno, pa nthawi yomwe amwasamutsa mokakamiza kuti azipita ku msasawu | omwe akukhala kunja kwa msasa wa Dzaleka achitilidwa ndi apolisi komanso a ku nthambi ya zolowa ndi zotuluka mdziko muno, pa nthawi yomwe amwasamutsa mokakamiza kuti azipita ku msasawu | Female | |
Nkhanzazi ndi monga kuwamenya, kuwalanda katundu komanso kutsekera ana mchitokosi cha apolisi. Nduna ya za chitetezo Cha m'dziko, Ken Zikhale Ng’oma yati anthu 300 amangidwa pa ntchitoyi | Nkhanzazi ndi monga kuwamenya, kuwalanda katundu komanso kutsekera ana mchitokosi cha apolisi. Nduna ya za chitetezo Cha m'dziko, Ken Zikhale Ng’oma yati anthu fili handiledi amangidwa pa ntchitoyi | Female | |
ndipo awatumiza ku Dzaleka posachedwapa. Komatu MHRC yati adindo akuyenera kulemekeza ufulu wa munthu aliyense pa nthawi yomwe akugwira ntchitoyi | ndipo awatumiza ku Dzaleka posachedwapa. Komatu emuetchialasi yati adindo akuyenera kulemekeza ufulu wa munthu aliyense pa nthawi yomwe akugwira ntchitoyi | Female | |
Anthu othawa kwawo pafupifupi 300 omwe amakhala kunja kwa msasa wa Dzaleka ali mchitokosi cha apolisi ku Lilongwe, atamangidwa pa nthawi yomwe apolisi amawathamangitsa kuti abwelere ku msasawu | Anthu othawa kwawo pafupifupi fili handiledi omwe amakhala kunja kwa msasa wa Dzaleka ali mchitokosi cha apolisi ku Lilongwe, atamangidwa pa nthawi yomwe apolisi amawathamangitsa kuti abwelere ku msasawu | Female | |
Boma likufuna kuti anthuwa, omwe ena mwa iwo amachita ntchito za malonda, abwelere komanso kumakakhala ku Dzaleka m'boma la Dowa monga mwa malamulo | Boma likufuna kuti anthuwa, omwe ena mwa iwo amachita ntchito za malonda, abwelere komanso kumakakhala ku Dzaleka m'boma la Dowa monga mwa malamulo | Female | |
Bomali linapereka mpaka pa 15 April chaka chino kuti anthuwa akhale atabwelera ku msasawu ndipo kupyolera apo ligwilitsa ntchito mphanvu zomwe pano zayamba kuchitika | Bomali linapereka mpaka pa fifitini epulo chaka chino kuti anthuwa akhale atabwelera ku msasawu ndipo kupyolera apo ligwilitsa ntchito mphanvu zomwe pano zayamba kuchitika | Female | |
Ngakhale boma likuchita izi, anthu ena akhala akutsutsana ndi ganizoli ponena kuti mwa njira ina, pali kuphwanya ufulu wa anthu othawa kwawo | Ngakhale boma likuchita izi, anthu ena akhala akutsutsana ndi ganizoli ponena kuti mwa njira ina, pali kuphwanya ufulu wa anthu othawa kwawo | Female | |
Bungwe lothandiza anthu la Malawi Red Cross Society (MRCS), lapereka zipangizo zosiyanasiyana ku ofesi ya zaumoyo m'boma la Blantyre zomwe zithandizire kulimbana ndi nthenda ya cholera | Bungwe lothandiza anthu la Malawi ledi khulosi sosayate (emualasiyesi), lapereka zipangizo zosiyanasiyana ku ofesi ya zaumoyo m'boma la Bulantaya zomwe zithandizire kulimbana ndi nthenda ya kolela | Female | |
Zipangizozi akuti zilimbikitse kuchepetsabe chiwelengero cha anthu omwe akudwala nthendayi, pomwe pano chikutsika | Zipangizozi akuti zilimbikitse kuchepetsabe chiwelengero cha anthu omwe akudwala nthendayi, pomwe pano chikutsika | Female | |
Poyankhula pa mwambo opereka zipangizozi, mlembi ku bungwe la MRCS, McBain Kanongodza wati bungwe lawo limazindikira zakufunika kwa thandizo ngati ili | Poyankhula pa mwambo opereka zipangizozi, mlembi ku bungwe la emualasiyesi, makibeni Kanongodza wati bungwe lawo limazindikira zakufunika kwa thandizo ngati ili | Female | |
ndipo lipitilira kuchilimika pofuna kuonetsetsa kuti anthu akuthandizidwa mu njira zosiyanasiyana monga za umoyo | ndipo lipitilira kuchilimika pofuna kuonetsetsa kuti anthu akuthandizidwa mu njira zosiyanasiyana monga za umoyo | Female | |
Bungwe la MRCS lapereka zipangizozi ndi thandizo lochokera ku bungwe la Qatar Red Crescent Society ndipo ndi la ndalama zokwana K180 million | Bungwe la emualasiyesi lapereka zipangizozi ndi thandizo lochokera ku bungwe la kata ledi kilesenti sosayate ndipo ndi la ndalama zokwana eitini miliyoni kwacha | Female | |
Pakadalipano, m'modzi mwa madotolo ku ofesi ya zaumoyo m'boma la Blantyre, Dr. Hawa Ntitimila ayamikira thandizoli lomwe akuti lafika pa nthawi yake | Pakadalipano, m'modzi mwa madotolo ku ofesi ya zaumoyo m'boma la Bulantaya, Dokota. Hawa Ntitimila ayamikira thandizoli lomwe akuti lafika pa nthawi yake | Female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.