audio audioduration (s) 1.12 18.5 | raw_text stringlengths 1 297 | normalized_text stringlengths 1 267 | gender stringclasses 16
values |
|---|---|---|---|
Mwa chitsanzo, a Timothy Mtambo, a Gospel Kazako komanso a Khumbize Kandodo Chiponda ndi a Lobin Lowe apitilira kukhala nduna za mgwirizano wa m'dziko, kufalitsa nkhani, umoyo komanso ulimi | Mwa chitsanzo, a Timofe Mtambo, a gosipelo Kazako komanso a Khumbize Kandodo Chiponda ndi a Lobini Lowe apitilira kukhala nduna za mgwirizano wa m'dziko, kufalitsa nkhani, umoyo komanso ulimi | Female | |
Pakadali pano, a Chakwera asankha a Sosten Gwengwe kukhala nduna ya za chuma kulowa m'malo mwa a Felix Mlusu omwe pano alibe unduna uli onse | Pakadali pano, a Chakwera asankha a Sositeni Gwengwe kukhala nduna ya za chuma kulowa m'malo mwa a Felikisi Mlusu omwe pano alibe unduna uli onse | Female | |
Mtsogoleriyu wasankhanso a Albert Mbawala kukhala nduna ya za migodi pamene a Ibrahim Matola akhala nduna ya za magetsi | Mtsogoleriyu wasankhanso a Albati Mbawala kukhala nduna ya za migodi pamene a Ibulahimu Matola akhala nduna ya za magetsi | Female | |
A Richard Chimwendo Banda tsopano ndi nduna ya za masewero, kulowa m'malo mwa a Ulemu Msungama pamene a Eisenhower Mkaka ndi nduna ya za chilengedwe | A litchadi Chimwendo Banda tsopano ndi nduna ya za masewero, kulowa m'malo mwa a Ulemu Msungama pamene a Esenihova Mkaka ndi nduna ya za chilengedwe | Female | |
kusinthana ndi a Nancy Tembo omwe tsopano akhale nduna ya za ubale wa dziko lino ndi maiko ena | kusinthana ndi a Nanse Tembo omwe tsopano akhale nduna ya za ubale wa dziko lino ndi maiko ena | Female | |
Mtsogoleriyu wasankhanso a Madalitso Kambauwa-Wirima kukhala wachiwiri kwa nduna ya za ulimi pamene a Harry Mkandawire ndi wachiwiri kwa nduna ya za chitetezo | Mtsogoleriyu wasankhanso a Madalitso Kambauwa-Wirima kukhala wachiwiri kwa nduna ya za ulimi pamene a Hale Mkandawire ndi wachiwiri kwa nduna ya za chitetezo | Female | |
Pakadali pano, unduna wa za chitetezo cha mziko uli m'manja mwa a Jean Sendeza, omwe m'mbuyomu anali wachiwiri kwa nduna ya za chitetezo | Pakadali pano, unduna wa za chitetezo cha mziko uli m'manja mwa a Jini Sendeza, omwe m'mbuyomu anali wachiwiri kwa nduna ya za chitetezo | Female | |
Mu mndandanda wa nduna za tsopanozi, a Chakwera abweretsanso unduna wa za madzi ndi ukhondo omwe nduna yake akhale a Abida Mia | Mu mndandanda wa nduna za tsopanozi, a Chakwera abweretsanso unduna wa za madzi ndi ukhondo omwe nduna yake akhale a Abida Miya | Female | |
Izitu ndi Zina mwa nduna zomwe a Chakwera asankha. Aka ndi kachiwiri kuti president Lazarus Chakwera asankhe nduna za boma pomwe anasankha nduna zake koyamba mchaka cha 2020 | Izitu ndi Zina mwa nduna zomwe a Chakwera asankha. Aka ndi kachiwiri kuti pulezidenti Lazalasi Chakwera asankhe nduna za boma pomwe anasankha nduna zake koyamba mchaka cha twente twente | Female | |
Ana awiri abanja limodzi kwa Bvumbwe boma la Thyolo amwalira ndipo mayi awo athyoka miyendo nyumba itawagwera Izizikutsatira mvula ya mphanvu yomwe ikugwa Madera ambiri mdziko muno | Ana awiri abanja limodzi kwa Bvumbwe boma la Thyolo amwalira ndipo mayi awo athyoka miyendo nyumba itawagwera Izizikutsatira mvula ya mphanvu yomwe ikugwa Madera ambiri mdziko muno | Female | |
Malipoti akuti nyumbayi yawagwera usiku wapitawu pomwe mayiyu pamodzi ndi anawa anali mtulo, kufikira pomwe anakwililika ndi njerwa za nyumbayi | Malipoti akuti nyumbayi yawagwera usiku wapitawu pomwe mayiyu pamodzi ndi anawa anali mtulo, kufikira pomwe anakwililika ndi njerwa za nyumbayi | Female | |
Malingana ndi yemwe watitumizira nkhaniyi, zinatengera anthu akufuna kwabwino omwe ataona ngoziyi anathamanga kukapulumusa anthuwa koma za chisoni nkuti anawa anali atamwalira ndipo mayiwa avulala miyendo | Malingana ndi yemwe watitumizira nkhaniyi, zinatengera anthu akufuna kwabwino omwe ataona ngoziyi anathamanga kukapulumusa anthuwa koma za chisoni nkuti anawa anali atamwalira ndipo mayiwa avulala miyendo | Female | |
Anthuwa ndi a mudzi mwa Kadambo mfumu yayikulu Bvumbwe boma la thyolo. A Chakwera ati alengeza nduna za tsopano m'masiku awiri akubwerawa | Anthuwa ndi a mudzi mwa Kadambo mfumu yayikulu Bvumbwe boma la thyolo. A Chakwera ati alengeza nduna za tsopano m'masiku awiri akubwerawa | Female | |
Iwo ati mu mndandanda wa nduna za tsopanowu simukhala nduna yakale ya za malo a Kezzie Msukwa omwe pakadali pano akuyankha milandu ya katangale | Iwo ati mu mndandanda wa nduna za tsopanowu simukhala nduna yakale ya za malo a Kezi Msukwa omwe pakadali pano akuyankha milandu ya katangale | Female | |
Ndipo kupatula nkhani ya maundunawa, a Chakwera ati achenjezanso mkulu wa bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu la ACB kaamba kosowa mwambo pa ntchito | Ndipo kupatula nkhani ya maundunawa, a Chakwera ati achenjezanso mkulu wa bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu la esibi kaamba kosowa mwambo pa ntchito | Female | |
A Chakwera apeleka chenjezoli patangopita tsiku limodzi lokha, pa masamba a mchezo patafalikira uthenga wina omwe uli ndi mau a a Chizuma omwe amayankhulana ndi munthu wina pa phone | A Chakwera apeleka chenjezoli patangopita tsiku limodzi lokha, pa masamba a mchezo patafalikira uthenga wina omwe uli ndi mau a a Chizuma omwe amayankhulana ndi munthu wina pa foni | Female | |
momwe ntchito za ACB zikuyendera. Pamenepa, mtsogoleri wa dziko linoyu wati sachotsa a Chizuma pa ntchito yawo ngakhale alakwira ena mwa malamulo a ntchito yawo | momwe ntchito za esibi zikuyendera. Pamenepa, mtsogoleri wa dziko linoyu wati sachotsa a Chizuma pa ntchito yawo ngakhale alakwira ena mwa malamulo a ntchito yawo | Female | |
A polisi ati akufunafuna a Bon Kalindo omwe akuti akuwaganizira kuti apalamula mlandu onyoza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera | A polisi ati akufunafuna a Boni Kalindo omwe akuti akuwaganizira kuti apalamula mlandu onyoza mtsogoleri wa dziko lino a Lazalasi Chakwera | Female | |
Malingana ndi chikalata chomwe apolisi atulusa, a Kalindo akuwaganizira kuti anapalamula mlandu-wu lachisanu mu mzinda wa Blantyre | Malingana ndi chikalata chomwe apolisi atulusa, a Kalindo akuwaganizira kuti anapalamula mlandu-wu lachisanu mu mzinda wa Bulantaya | Female | |
pa nthawi yomwe amasogolera a Malawi kuchita zionesero zosonyesa ku kwiya ndi ulamuliro wa a Chakwera | pa nthawi yomwe amasogolera a Malawi kuchita zionesero zosonyesa ku kwiya ndi ulamuliro wa a Chakwera | Female | |
Mneneri wa apolisi m'dziko muno James Kadadzera watsimikiza za kusakidwa kwa a Kalindo omwe pakadali pano sakuziwa komwe ali | Mneneri wa apolisi m'dziko muno Jemusi Kadadzera watsimikiza za kusakidwa kwa a Kalindo omwe pakadali pano sakuziwa komwe ali | Female | |
A kadadzera auza a Bon Kalindo kuti akazipereke okha ku polisi yomwe ali nayo pafupi. Pakadali pano ma lamya onse a Kalindo ndi ozima | A kadadzera auza a Boni Kalindo kuti akazipereke okha ku polisi yomwe ali nayo pafupi. Pakadali pano ma lamya onse a Kalindo ndi ozima | Female | |
ndipo ma repoti ena pa ma samba a nchezo akusonyeza kuti apolisi ambiri omwe anali ndi mfuti anapita ku nyumba kwawo komwe sanawapeze | ndipo ma repoti ena pa ma samba a nchezo akusonyeza kuti apolisi ambiri omwe anali ndi mfuti anapita ku nyumba kwawo komwe sanawapeze | Female | |
Anyamata awiri ogulitsa mankhwala a msikizi ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre akunthana modetsa nkhawa kutsatira kunyozana komwe kunabuka kasitomala wina atagula mmodzi mwa iwo mankhwala-wa ndi kusiya winayo | Anyamata awiri ogulitsa mankhwala a msikizi ku Ndirande mu mzinda wa Bulantya akunthana modetsa nkhawa kutsatira kunyozana komwe kunabuka kasitomala wina atagula mmodzi mwa iwo mankhwala-wa ndi kusiya winayo | Female | |
Nkhaniyi ikuti kasitomala-yu anaimitsa mmodzi mwa anayamata-wa kuti agule mankhwala a msikizi-wa koma onse anaima ndi chiyembekezo choti agulidwa malonda awowa | Nkhaniyi ikuti kasitomala-yu anaimitsa mmodzi mwa anayamata-wa kuti agule mankhwala a msikizi-wa koma onse anaima ndi chiyembekezo choti agulidwa malonda awowa | Female | |
Pamenepa munthuyu anagula mmodzi mwa iwo mankhwala-wa yemwe anayamba kunyoza mnzakeyu ponena kuti malonda ake sakugudwa poyelekeza ndi iyeyo | Pamenepa munthuyu anagula mmodzi mwa iwo mankhwala-wa yemwe anayamba kunyoza mnzakeyu ponena kuti malonda ake sakugudwa poyelekeza ndi iyeyo | Female | |
Apa mkwiyo unamanga nthenje mwa onyezedwayu yemwe anayamba kuzivumbulutsa zibakera ndipo apa ndi pomwe ndewu inabuka | Apa mkwiyo unamanga nthenje mwa onyezedwayu yemwe anayamba kuzivumbulutsa zibakera ndipo apa ndi pomwe ndewu inabuka | Female | |
Malipoti akuti zinatengera anthu ena akufuna kwabwino kuleletsa ndewu-yo komatu ena atafa ndi phwete ponena kuti anyamata-wa amenyana pa chifukwa chopanda pake | Malipoti akuti zinatengera anthu ena akufuna kwabwino kuleletsa ndewu-yo komatu ena atafa ndi phwete ponena kuti anyamata-wa amenyana pa chifukwa chopanda pake | Female | |
A Bon Kalindo omwe akhala akutsogolera zionetsero zosonyeza kusakondwa ndi boma la mgwirizano wa Tonse ati apitilira ndi ganizo lawo lotsogoleri anthu kuseka Chipata cha Chingeni ku Ntcheu | A Boni Kalindo omwe akhala akutsogolera zionetsero zosonyeza kusakondwa ndi boma la mgwirizano wa Tonse ati apitilira ndi ganizo lawo lotsogoleri anthu kuseka Chipata cha Chingeni ku Ntcheu | Female | |
Iwo auza wailesi ina m’dziko muno kuti ndi zosamveka kuti munthu azilipira pa zipatazi ulendo ulionse akudutsa, ponena kuti boma likanakhalazikitsa kuti munthu azilipira Kamodzi chabe | Iwo auza wailesi ina m’dziko muno kuti ndi zosamveka kuti munthu azilipira pa zipatazi ulendo ulionse akudutsa, ponena kuti boma likanakhalazikitsa kuti munthu azilipira Kamodzi chabe | Female | |
Komatu mneneri wa boma, a Gospel Kazako ati zomwe a Kalindo akufuna kuchita ndi zongofuna kulimbana ndi boma pa ndale chabe osati kumenyera ufulu wa anthu | Komatu mneneri wa boma, a Gosipelo Kazako ati zomwe a Kalindo akufuna kuchita ndi zongofuna kulimbana ndi boma pa ndale chabe osati kumenyera ufulu wa anthu | Female | |
Apolisi m’boma la Mulanje ati ayamba kufufuza anthu omwe achita chipongwe bambo wa zaka 23, Thomson Tomasi | Apolisi m’boma la Mulanje ati ayamba kufufuza anthu omwe achita chipongwe bambo wa zaka twente fili, Thomusoni Tomasi | Female | |
pomudula ziwalo zobisika m’bandakucha wa lamulungu lapitali. Mneneri wa polisi m’bomali, Gresham Ngwira wati Tomasi anachitidwa za upanduzi pafupi ndi msika wa Nkando wa m’bamali | pomudula ziwalo zobisika m’bandakucha wa lamulungu lapitali. Mneneri wa polisi m’bomali, Gileshamu Ngwira wati Tomasi anachitidwa za upanduzi pafupi ndi msika wa Nkando wa m’bamali | Female | |
Malingana ndi a Ngwira, mkuluyu anali magazi okha-okha zomwe zinachtiitsa kuti amutengere ku chipatala cha Mulanje | Malingana ndi a Ngwira, mkuluyu anali magazi okha-okha zomwe zinachtiitsa kuti amutengere ku chipatala cha Mulanje | Female | |
komwe anamupambanitsira ku chipatala cha Queen Elizabeth mu mzinda wa Blantyre komwe akulandira thandizo la mankhwala | komwe anamupambanitsira ku chipatala cha Kwini elizabefi mu mzinda wa Bulantaya komwe akulandira thandizo la mankhwala | Female | |
Chipani cha Malawi Congress (MCP) chati chikulirabe imfa ya yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wake, mchigawo cha kum’mwera malemu Sidik Mia yemwe anamwalira ndi mliri wa COVID-19 | Chipani cha Malawi kongelesi ( Emusipi ) chati chikulirabe imfa ya yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wake, mchigawo cha kum’mwera malemu Sidiki Miya yemwe anamwalira ndi mliri wa Kovidi-naintini | Female | |
Izitu ndi malingana ndi mneneri wa chipanichi, m’busa Maurice Munthali yemwe wati ichi ndi chifukwa chake kufikira pano, chipanichi sichinapeze mulowa m’malo wa a Mia | Izitu ndi malingana ndi mneneri wa chipanichi, m’busa Molisi Munthali yemwe wati ichi ndi chifukwa chake kufikira pano, chipanichi sichinapeze mulowa m’malo wa a Mia | Female | |
Komabe, mneneri wa MCP-yu wati tsogolo la yemwe atenge m’pandowu lidziwika pa msonkhano wake waukulu omwe uchitike mtsogolomu ngakhale kuti sizikudziwika kuti uchitika liti | Komabe, mneneri wa emusipi-yu wati tsogolo la yemwe atenge m’pandowu lidziwika pa msonkhano wake waukulu omwe uchitike mtsogolomu ngakhale kuti sizikudziwika kuti uchitika liti | Female | |
Pafupi-fupi chaka chadutsa tsopano kuchokera pomwe a Sidik Mia omwenso anali nduna ya za maulendo ndi ntchito za mtengatenga anamwalira | Pafupi-fupi chaka chadutsa tsopano kuchokera pomwe a Sidiki Miya omwenso anali nduna ya za maulendo ndi ntchito za mtengatenga anamwalira | Female | |
MacDonald Manase wa m’boma la Chiradzulu amugamula kukakhala ku ndende kwa zaka 8 ndi miyezi khumi atapezeka olakawa pa mlandu opezeka ku Phiri ndi mtsikana wina koma onse ali buno bwamuse | Makidonadi Manase wa m’boma la Chiradzulu amugamula kukakhala ku ndende kwa zaka eiti ndi miyezi khumi atapezeka olakawa pa mlandu opezeka ku Phiri ndi mtsikana wina koma onse ali buno bwamuse | Female | |
Yemwe amaimira boma pa mlanduwu, Witson Nyalugwe anauza bwalolo kuti mkuluyu anapalamula mlanduwu pa 31 October chaka chatha pa mudzi pa Mkwanda mfumu yaikulu Likoswe m’boma lomweli la Chiradzulu | Yemwe amaimira boma pa mlanduwu, Witisoni Nyalugwe anauza bwalolo kuti mkuluyu anapalamula mlanduwu pa fete wani okutoba chaka chatha pa mudzi pa Mkwanda mfumu yaikulu Likoswe m’boma lomweli la Chiradzulu | Female | |
Malingana ndi Nyalugwe, Manase atapezeka ndi mtsikana-yu yemwe akuti ali ndi vuto la mu ubongo, anthu anamugwira ndi kukamupeleka ku polisi komwe anamutsegulira mlandu | Malingana ndi Nyalugwe, Manase atapezeka ndi mtsikana-yu yemwe akuti ali ndi vuto la mu ubongo, anthu anamugwira ndi kukamupeleka ku polisi komwe anamutsegulira mlandu | Female | |
Bambo wazaka 37 zakubadwa, Geoffrey Banda, wamwalira m’boma la Kasungu atawombedwa ndi mphezi. Ofalitsa nkhani za apolisi m’bomali, Joseph Kachikho | Bambo wazaka fete seveni zakubadwa, JofuleBanda, wamwalira m’boma la Kasungu atawombedwa ndi mphezi. Ofalitsa nkhani za apolisi m’bomali, Jozefe Kachikho | Female | |
watsimikiza za ngozi-yi yomwe wati yachitika usiku wapitawu. Malingana ndi a Kachikho, malemu Banda anaombedwa ndi mpheziyi | watsimikiza za ngoziyi yomwe wati yachitika usiku wapitawu. Malingana ndi a Kachikho, malemu Banda anaombedwa ndi mpheziyi | Female | |
pa nthawi yomwe amakonza nyumba yawo panja pa nyumba yawo. Geoffrey Banda, anali a m’mudzi mwa Lembanyama m’dera la mfumu yaikulu Kawamba m’ boma lomweli la Kasungu | pa nthawi yomwe amakonza nyumba yawo panja pa nyumba yawo. Jofule Banda, anali a m’mudzi mwa Lembanyama m’dera la mfumu yaikulu Kawamba m’ boma lomweli la Kasungu | Female | |
Thupi la Anne Muluzi yemwe anali mkazi wa mtsogoleri opuma wa dziko lino, Bakili Muluzi liikidwa m’manda lachinai Sabata ino | Thupi la Anne Muluzi yemwe anali mkazi wa mtsogoleri opuma wa dziko lino, Bakili Muluzi liikidwa m’manda lachinai Sabata ino | Female | |
Izitu ndi malingana ndi kalata yomwe mlembi mu ofesi ya mtsogoleri ndi nduna, Zangazanga Chikhosi watulutsa yomwe yatinso mwambo oika m’manda thupili uchitika motsogozedwa ndi asilikali | Izitu ndi malingana ndi kalata yomwe mlembi mu ofesi ya mtsogoleri ndi nduna, Zangazanga Chikhosi watulutsa yomwe yatinso mwambo oika m’manda thupili uchitika motsogozedwa ndi asilikali | Female | |
monga momwe mtsogoleri wa dziko lino, a Lazarus Chakwera alamulira. Mai Muluzi anamwalira Sabata yatha pa chipatala cha Aga Khan | monga momwe mtsogoleri wa dziko lino, a Lazalasi Chakwera alamulira. Mai Muluzi anamwalira Sabata yatha pa chipatala cha Aga Khani | Female | |
cha m’dziko la Kenya komwe amalandira thandizo la mankhwala ku nthenda ya cancer. Mtsogoleri wa kale wa dziko lino, Peter Mutharika komanso mtsogoleri ochita | cha m’dziko la Kenya komwe amalandira thandizo la mankhwala ku nthenda ya Khansa. Mtsogoleri wa kale wa dziko lino, Pita Mutharika komanso mtsogoleri ochita | Female | |
Lazarus Chakwera ndi akulu-akulu ena, akuyembekezereka kukakhala nawo pa mwambowu | Lazalasi Chakwera ndi akulu-akulu ena, akuyembekezereka kukakhala nawo pa mwambowu | Female | |
M’busa wina m’dziko la Ghana wadabwitsa anthu atalamula akhiristu ake a akazi kuti avule zomvala zawo zonse ndi kuti awasambitse ngati njira imodzi yowachosera uchimo | M’busa wina m’dziko la Gana wadabwitsa anthu atalamula akhiristu ake a akazi kuti avule zomvala zawo zonse ndi kuti awasambitse ngati njira imodzi yowachosera uchimo | Female | |
Kenema yemwe akuzungulira pa matsamba a mchezo apa Internet, akuonetsa ena mwa amayiwa ali chibadwire uku Mtumiki wa Mulunguyu akuwasambitsa pa guwa | Kenema yemwe akuzungulira pa matsamba a mchezo apa Intaneti, akuonetsa ena mwa amayiwa ali chibadwire uku Mtumiki wa Mulunguyu akuwasambitsa pa guwa | Female | |
Pomwe zimachitika izi mkuti a akhiristu amuna, omwe ena mwa iwo ndi azimuna awo a amayiwa, ali chilili kuyimba nyimbo kwinaku akuonelera mwambo odabwitsau | Pomwe zimachitika izi mkuti a akhiristu amuna, omwe ena mwa iwo ndi azimuna awo a amayiwa, ali chilili kuyimba nyimbo kwinaku akuonelera mwambo odabwitsau | Female | |
Izi zachitika usiku wapa 31 December, pa mapemphero apadera olowera m'chaka chasopano cha 2022 | Izi zachitika usiku wapa fete wani disemba, pa mapemphero apadera olowera m'chaka chasopano cha twente twente thu | Female | |
Anthu ochuluka pa tsamba la mchezo la Facebook adzudzula kolimba nduna ya zofalitsa a Gospel Kazako pa uthenga omwe alemba pa tsambali | Anthu ochuluka pa tsamba la mchezo la Fesibuku adzudzula kolimba nduna ya zofalitsa a Gosipelo Kazako pa uthenga omwe alemba pa tsambali | Female | |
opempha amalawi kuti adekhe ponena kuti Mavuto omwe akukumana nawo ndi a ka nthawi kochepa chabe. Uwu ndi uthenga oyamba mchaka chino cha 2022 kuchokera kwa ndunayi kupita kwa amalawi | opempha amalawi kuti adekhe ponena kuti Mavuto omwe akukumana nawo ndi a ka nthawi kochepa chabe. Uwu ndi uthenga oyamba mchaka chino cha twente twente thu kuchokera kwa ndunayi kupita kwa amalawi | Female | |
omwe kwambiri ukulunjika kuti boma la mgwirizano wa Tonse likuzindikira za kuwawa komwe anthu akumva m’magawo a za umoyo, chuma ndi ena | omwe kwambiri ukulunjika kuti boma la mgwirizano wa Tonse likuzindikira za kuwawa komwe anthu akumva m’magawo a za umoyo, chuma ndi ena | Female | |
Komatu ambiri mwa anthu omwe ndi opitilira 11, 000 omwe aikira ndemanga pa mawu a ndunayi, aonetsa kukhumudwa komanso mkwiyo ndi izi | Komatu ambiri mwa anthu omwe ndi opitilira leveni sauzande omwe aikira ndemanga pa mawu a ndunayi, aonetsa kukhumudwa komanso mkwiyo ndi izi | Female | |
pomwe akuti ndi zokaikitsa ngati kusintha komwe kumayenera kuoneka m’dziko muno kuonekenso. Mtsinje wa Nasolo ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre wasefukira kaamba ka mvula yomwe yagwa masana a lero | pomwe akuti ndi zokaikitsa ngati kusintha komwe kumayenera kuoneka m’dziko muno kuonekenso. Mtsinje wa Nasolo ku Ndirande mu mzinda wa Bulantaya wasefukira kaamba ka mvula yomwe yagwa masana a lero | Female | |
Pa nkhani ya ndondomeko yothandiza kupewa kufala kwa mliri, komitiyi yalengeza kuti chiwelengero cha anthu osankhana pamodzi mnyumba achitsitsa kufika pa 100 | Pa nkhani ya ndondomeko yothandiza kupewa kufala kwa mliri, komitiyi yalengeza kuti chiwelengero cha anthu osankhana pamodzi mnyumba achitsitsa kufika pa wani handiledi | Female | |
pamene onse omwe azisonkhana panja sakuyenera kumapitilira 250. Izi akuti ziyamba kugwira ntchito lolemba likudzali | pamene onse omwe azisonkhana panja sakuyenera kumapitilira thu handiledi andi fifite. Izi akuti ziyamba kugwira ntchito lolemba likudzali | Female | |
Komiti ya mtsogoleri wa dziko pa mliri wa COVID-19 yalengeza kuti boma liri ndi malingaliro ofuna kuyamba kukakamiza onse ogwira ntchito m'boma kuti abayitse katemera woteteza ku mliriwu | Komiti ya mtsogoleri wa dziko pa mliri wa kovidi-naintini yalengeza kuti boma liri ndi malingaliro ofuna kuyamba kukakamiza onse ogwira ntchito m'boma kuti abayitse katemera woteteza ku mliriwu | Female | |
Izi zalengezedwa pa msonkhano wa atolankhani ku Lilongwe. Zipani zotsutsa boma za DPP ndi UDF | Izi zalengezedwa pa msonkhano wa atolankhani ku Lilongwe. Zipani zotsutsa boma za Dipipi ndi yudiefu | Female | |
lero zichititsa msonkhano wa atolankhani patsogolo pa msonkhano wake wa ndale omwe zochititse lamulungu likubwerali | lero zichititsa msonkhano wa atolankhani patsogolo pa msonkhano wake wa ndale omwe zochititse lamulungu likubwerali | Female | |
Mneneri wa chipani cha DPP, a Shadreck Namalomba, komanso a Yunus, komanso a Yusuf Mwawa omwe amayankhulira UDF ndi ena mwa anthu omwe ayankhule atolankhani pa msonkhanowu | Mneneri wa chipani cha Dipipi, a Shadileki Namalomba, komanso a Yunusi, komanso a Yusufu Mwawa omwe amayankhulira Yudiefu ndi ena mwa anthu omwe ayankhule atolankhani pa msonkhanowu | Female | |
Akuluakulu a zipani ziwirizi komanso atolankhani kuchokera ku nyumba zosiyanasiyana zofalitsa nkhani afika ku malo omwe kuchitikire msonkhanowu ku Naperi mu mzinda wa Blantyre | Akuluakulu a zipani ziwirizi komanso atolankhani kuchokera ku nyumba zosiyanasiyana zofalitsa nkhani afika ku malo omwe kuchitikire msonkhanowu ku Naperi mu mzinda wa Bulantaya | Female | |
Komiti ya mtsogoleri wa dziko lino pa mliri wa COVID-19 lero ikulengeza ndondomeko za tsopano zopewera mliriwu pomwe gawo lachinayi labuka m’dziko muno | Komiti ya mtsogoleri wa dziko lino pa mliri wa kovidi - naintini lero ikulengeza ndondomeko za tsopano zopewera mliriwu pomwe gawo lachinayi labuka m’dziko muno | Female | |
Komitiyi inakumana dzulo mu mzinda wa Lilongwe komwe mwa zina inakambirana zomwe ziyenera kuchitika pakadali pano pofuna kulimbana ndi gawoli | Komitiyi inakumana dzulo mu mzinda wa Lilongwe komwe mwa zina inakambirana zomwe ziyenera kuchitika pakadali pano pofuna kulimbana ndi gawoli | Female | |
Ndondomekozi akuzilengeza kudzera pa msonkhano wa atolankhani omwe ukuchitikira mu mzinda wa Lilongwe | Ndondomekozi akuzilengeza kudzera pa msonkhano wa atolankhani omwe ukuchitikira mu mzinda wa Lilongwe | Female | |
Katundu wa nkhaninkhani komanso nyumba ndi makachisi zaonongeka m'midzi ina ya m'boma la Chikwawa kutsatira Mvula ya mphanvu yomwe yagwa m'bomalo lero | Katundu wa nkhaninkhani komanso nyumba ndi makachisi zaonongeka m'midzi ina ya m'boma la Chikwawa kutsatira Mvula ya mphanvu yomwe yagwa m'bomalo lero | Female | |
M'modzi mwa anthu omwe aona izi zikuchitika, Edith Mvula watiuza kuti umodzi mwa midziyi ndi wa Chikhambi omwe uli mdera la mfumu yaikulu Kasisi | M'modzi mwa anthu omwe aona izi zikuchitika, Edifi Mvula watiuza kuti umodzi mwa midziyi ndi wa Chikhambi omwe uli mdera la mfumu yaikulu Kasisi | Female | |
Kuonjezera apo, Edith akutinso pali nkhawa yoti mwana wina wavulala mtengo wa malambe utagwera nyumba yomwe anabisala kuthawa mvulayi Tikupatsireni zambiri za nkhaniyi mu nkhani zathu zotsatira | Kuonjezera apo, Edifi akutinso pali nkhawa yoti mwana wina wavulala mtengo wa malambe utagwera nyumba yomwe anabisala kuthawa mvulayi Tikupatsireni zambiri za nkhaniyi mu nkhani zathu zotsatira | Female | |
Patangopita mphindi zochepa chabe a Bon Kalindo atatulutsidwa pa bail mlandu okhuza kufalitsa nkhani za bodza, apolisi amumanganso mkuluyu pa mlandu omwe akumuganizira kuti anaonongetsa katundu | Patangopita mphindi zochepa chabe a Boni Kalindo atatulutsidwa pa belo mlandu okhuza kufalitsa nkhani za bodza, apolisi amumanganso mkuluyu pa mlandu omwe akumuganizira kuti anaonongetsa katundu | Female | |
A Kalindo akuwaganizira kuti anaonongetsa katunduyu pa zionetsero zomwe anatsogolera anthu mu mzinda wa Lilongwe sabata zingapo zapitazo | A Kalindo akuwaganizira kuti anaonongetsa katunduyu pa zionetsero zomwe anatsogolera anthu mu mzinda wa Lilongwe sabata zingapo zapitazo | Female | |
Pakadali pano, a Kalindo awasamutsa ku polisi ya Zomba ndipo tsopano akupita nawo ku polisi ya Lilongwe | Pakadali pano, a Kalindo awasamutsa ku polisi ya Zomba ndipo tsopano akupita nawo ku polisi ya Lilongwe | Female | |
Bungwe la Blantyre Water Board lapereka mphoto kwa ena mwa makasitomala ake omwe akuti akhala akudziwitsa bungweli | Bungwe la Bulantaya wota bodi lapereka mphoto kwa ena mwa makasitomala ake omwe akuti akhala akudziwitsa bungweli | Female | |
Bungwe la Blantyre Water Board lapereka mphoto kwa ena mwa makasitomala ake omwe akuti akhala akudziwitsa bungweli | Bungwe la Bulantaya wota bodi lapereka mphoto kwa ena mwa makasitomala ake omwe akuti akhala akudziwitsa bungweli | Female | |
za mavuto osiyanasiyana okhuza madzi omwe amakhala akuchita ku Madera awo | za mavuto osiyanasiyana okhuza madzi omwe amakhala akuchita ku Madera awo | Female | |
Bungweli lapeleka mphoto kwa a Lucius Kamoto a ku Chilobwe komanso banja la bambo ndi Mai Luke a ku Bangwe | Bungweli lapeleka mphoto kwa a Lucius Kamoto a ku Chilobwe komanso banja la bambo ndi Mai Luke a ku Bangwe | Female | |
omwe mwa zina akhala akudziwitsa bungweli ngati mapaipi a madzi aphulika, ngati madzi asiya komanso ngati anthu ena akuba madzi | omwe mwa zina akhala akudziwitsa bungweli ngati mapaipi a madzi aphulika, ngati madzi asiya komanso ngati anthu ena akuba madzi | Female | |
Apa, Blantyre water board kudzera mwa mneneri wake Evelyn Khonje yemwe anatsogolera mwambo opeleka mphotowu | Apa, Bulantaya wota bodi kudzera mwa mneneri wake Evelyn Khonje yemwe anatsogolera mwambo opeleka mphotowu | Female | |
walangiza anthu ena kutengera chitsanzo cha a Kamoto komanso bambo ndi mai Luke pofuna kuthana ndi mavuto okhuza kapelekedwe ka madzi mu mzinda wa Blantyre ndi Madera ozungulira | walangiza anthu ena kutengera chitsanzo cha a Kamoto komanso bambo ndi mai Luka pofuna kuthana ndi mavuto okhuza kapelekedwe ka madzi mu mzinda wa Bulantaya ndi Madera ozungulira | Female | |
Anthu okwiya ku Dedza amenya ndi kupha komanso kuotcha thupi la bambo wa zaka 64, Lawirani Paul Shadreck pa nkhani za ufiti | Anthu okwiya ku Dedza amenya ndi kupha komanso kuotcha thupi la bambo wa zaka sikisite folo, Lawirani Po Shadileki pa nkhani za ufiti | Female | |
Malipoti akuti anthuwa anachita izi kutsatira imfa ya mzukulu wake wa bamboyu yemwe anagwa mu mtengo ndi kukafikira mu chitsime momwe anamwalilira kaamba kobanika popuma | Malipoti akuti anthuwa anachita izi kutsatira imfa ya mzukulu wake wa bamboyu yemwe anagwa mu mtengo ndi kukafikira mu chitsime momwe anamwalilira kaamba kobanika popuma | Female | |
Komabe, achibale ena sanakhulupilire kuti imfa ya mwanayu inali ngozi chabe koma kuti a Shadreck ndi omwe anamulodza poonjezera kuti zotsatira za chipatala zomwe zinaonetsa kuti mwanayu anamwalira kaamba kobanika zinali zabodza | Komabe, achibale ena sanakhulupilire kuti imfa ya mwanayu inali ngozi chabe koma kuti a Shadileki ndi omwe anamulodza poonjezera kuti zotsatira za chipatala zomwe zinaonetsa kuti mwanayu anamwalira kaamba kobanika zinali zabodza | Female | |
Pamenepa, anthu anagwira malemu Shadreck yemwenso anali mfumu yaing’ono Kadzabwani ndi kuyamba kumumenya mpaka kumupha kenako ndi kuotcha thupi lake | Pamenepa, anthu anagwira malemu Shadileki yemwenso anali mfumu yaing’ono Kadzabwani ndi kuyamba kumumenya mpaka kumupha kenako ndi kuotcha thupi lake | Female | |
Pakadali pano, wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Dedza, Cassim Manda watiuza kuti apolisi atsekera mchitokosi Makolo ake a mwanayu | Pakadali pano, wachiwiri kwa mneneri wa polisi ya Dedza, kasimu Manda watiuza kuti apolisi atsekera mchitokosi Makolo ake a mwanayu | Female | |
omwe akuganizilidwa kuti akukhuzidwa kwambiri ndi za mtopolazi pomwe kafukufuku ofuna kupeza anthu ena okhuzidwa ali mkati | omwe akuganizilidwa kuti akukhuzidwa kwambiri ndi za mtopolazi pomwe kafukufuku ofuna kupeza anthu ena okhuzidwa ali mkati | Female | |
Mkulu wa bungwe lomenyera ufulu wa anthu ogula katundu la CAMA, John Kapito wadzudzula bungwe la Blantyre Water Board | Mkulu wa bungwe lomenyera ufulu wa anthu ogula katundu la KAMA, Joni Kapito wadzudzula bungwe la Bulantaya wota bodi | Female | |
kaamba kopanga mapulani a momwe ligwilire ntchito zake mu zaka zisanu zikubwerazi koma osafunsa maganizo a makasitomala ake | kaamba kopanga mapulani a momwe ligwilire ntchito zake mu zaka zisanu zikubwerazi koma osafunsa maganizo a makasitomala ake | Female | |
A Kapito ati izi zimachititsa kuti kampani komanso mabungwe azichita zinthu zomwe ndi zosakomera makasitomala awo kaamba koti sadziwa zimene anthuwo akufuna | A Kapito ati izi zimachititsa kuti kampani komanso mabungwe azichita zinthu zomwe ndi zosakomera makasitomala awo kaamba koti sadziwa zimene anthuwo akufuna | Female | |
Kapena tinene kuti alipo yemwe anafunsidwa maganizo apa ndi Blantyre Water Board isanapange strategic plan iyi Mwaonatu, limeneli ndi vuto lalikulu lomwe tili nalo mu kampani zambiri, atero a Kapito | Kapena tinene kuti alipo yemwe anafunsidwa maganizo apa ndi Bulantaya wota bodi isanapange sitiletejiki pulani iyi, Mwaonatu, limeneli ndi vuto lalikulu lomwe tili nalo mu kampani zambiri, atero a Kapito | Female | |
Pali malipoti oti anthu anai athamangira nawo ku chipatala cha Queen Elizabeth Central kutsatira kuvulala pa ngozi ya moto | Pali malipoti oti anthu anai athamangira nawo ku chipatala cha kwini elizabefi sentilo kutsatira kuvulala pa ngozi ya moto | Female | |
yomwe yachitika pa kampani yopanga machesi ya Leopard Matches 2018 Limited mu mzinda wa Blantyre | yomwe yachitika pa kampani yopanga machesi ya Leopadi Machesi twente eitini limited mu mzinda wa Bulantaya | Female | |
Motowu omwe kufikira pano chomwe chayambitsa sichikudziwika watentha kampani ya Leopard Matches komanso wakhuza kampani Zina zoyandikana nawo | Motowu omwe kufikira pano chomwe chayambitsa sichikudziwika watentha kampani ya Leopadi Machesi komanso wakhuza kampani Zina zoyandikana nawo | Female | |
monga Industrial Engineering, Meatco komanso Eshani Products Limited. Pakadali pano, akatswiri ozimitsa achilimika kuti athane ndi motowu ngakhale ukupitilirabe kuyaka | monga indasitiliyo injiniyaling’i, mitiko komanso Eshani Pulodakitsi Limitedi. Pakadali pano, akatswiri ozimitsa achilimika kuti athane ndi motowu ngakhale ukupitilirabe kuyaka | Female | |
Bungwe lopopa ndi kugulitsa madzi la Blantyre Water Board lero likhazikitsa ndondomeko ya momwe ligwilire ntchito zake strategic plan pa chingerezi ya zaka pafupifupi zisanu zikubwerazi | Bungwe lopopa ndi kugulitsa madzi la Bulantaya wota bodi lero likhazikitsa ndondomeko ya momwe ligwilire ntchito zake sitiletejiki pulani pa chingerezi ya zaka pafupifupi zisanu zikubwerazi | Female | |
Ofalitsa nkhani ku bungweli, Evelyn Khonje watiuza kuti mwambo okhazikitsa ndondomekozi uchitikira mu mzinda wa Blantyre | Ofalitsa nkhani ku bungweli, Evelini Khonje watiuza kuti mwambo okhazikitsa ndondomekozi uchitikira mu mzinda wa Bulantaya | Female | |
Malingana ndi Mai Khonje, pa mwambowu pakhalanso nduna ya za Chilengedwe mai Nancy Tembo ngati mlendo olemekezeka ndi anthu ena | Malingana ndi Mai Khonje, pa mwambowu pakhalanso nduna ya za Chilengedwe mai Nanse Tembo ngati mlendo olemekezeka ndi anthu ena | Female | |
Ndondomekoyi yomwe ndi ya zaka za pakati pa 2020 mpaka 2025 ionetsa momwe Blantyre Water Board itumikilire makasitomala ake | Ndondomekoyi yomwe ndi ya zaka za pakati pa twente twente mpaka twente twente faifi ionetsa momwe bulantaya wota bodi itumikilire makasitomala ake | Female |
Subsets and Splits
No community queries yet
The top public SQL queries from the community will appear here once available.