audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
akafuna kupeza madzi a ukhondo ngakhale Mabungwewa amakhala akudziwa kale za Mavuto omwe alipo
akafuna kupeza madzi a ukhondo ngakhale Mabungwewa amakhala akudziwa kale za Mavuto omwe alipo
Female
Iwo amayankhula izi lero mu mzinda wa Blantyre pa mwambo omwe mabungwe-wa amasainira mgwirizano ndi bungwe la CAMA omwe cholinga chake ndi kufuna kuonetsetsa kuti ufulu wa makasitomala ukulemezekedwa
Iwo amayankhula izi lero mu mzinda wa Bulantaya pa mwambo omwe mabungwe-wa amasainira mgwirizano ndi bungwe la KAMA omwe cholinga chake ndi kufuna kuonetsetsa kuti ufulu wa makasitomala ukulemezekedwa
Female
Malingana ndi a Kapito, ngati mabungwe opopa ndi kugulitsa madziwa aziphwanya mgwirizanowu, bungwe la CAMA lizichitapo kanthu mwa nsanga
Malingana ndi a Kapito, ngati mabungwe opopa ndi kugulitsa madziwa aziphwanya Mgwirizanowu, bungwe la KAMA lizichitapo kanthu mwa nsanga
Female
Ndipo m’mau ake, mkulu wa mgwirizano wa mabungwe opopa ndi kugulitsa madzi la Water Services Association of Malawi (WASAMA)
Ndipo m’mau ake, mkulu wa mgwirizano wa mabungwe opopa ndi kugulitsa madzi la Wota sevisezi asosiyeshoni ofu Malawi (WASAMA)
Female
Robert Hanjahanja wavomereza za mavuto omwe bungwe la CAMA lanena koma wati zinthu zisintha
Robati Hanjahanja wavomereza za mavuto omwe bungwe la KAMA lanena koma wati zinthu zisintha
Female
A Hanjahanja ati Mabungwewa amalephera kutumikira anthu kaamba ka Mavuto a chuma koma pano zinthu zisintha kaamba koti aloledwa kukweza mitengo ya madzi
A Hanjahanja ati Mabungwewa amalephera kutumikira anthu kaamba ka Mavuto a chuma koma pano zinthu zisintha kaamba koti aloledwa kukweza mitengo ya madzi
Female
Ena mwa mabungwe omwe asainira nawo mgwirizanowu ndi a Blantyre Water Board , Lilongwe Water Board komanso Northern Region Water Board
Ena mwa mabungwe omwe asainira nawo mgwirizanowu ndi a Bulantaya wota bodi , Lilongwe wota bodi komanso novena lijoni wota bodi
Female
Apolisi mu mzinda wa Blantyre lero ayamba kugwira komanso kutsekera mchitokosi anyamata oitanira minibus
Apolisi mu mzinda wa Bulantaya lero ayamba kugwira komanso kutsekera mchitokosi anyamata oitanira minibasi
Female
patapita Sabata imodzi boma litalengeza kuti likufuna kuchotsa anyamatawa m’miseu ndi malo ena okwelera galimoto
patapita Sabata imodzi boma litalengeza kuti likufuna kuchotsa anyamatawa m’miseu ndi malo ena okwelera galimoto
Female
Mneneri wa polisi ya Blantyre, Peter Mchiza wati ntchitoyi yayambira pa malo okwelera bus a Wenela ndipo ipitilira mpaka anyamata-wa atasiyiratu izi
Mneneri wa polisi ya Bulantaya, Pita Mchiza wati ntchitoyi yayambira pa malo okwelera basi a Wenela ndipo ipitilira mpaka anyamata-wa atasiyiratu izi
Female
A Mchiza ati apolisi agwira anyamata khumi ndi asanu omwe awatengere ku bwalo la milandu komwe akayankhe milandu yoitanira galimoto zomwe ndi zosemphana ndi malamulo
A Mchiza ati apolisi agwira anyamata khumi ndi asanu omwe awatengere ku bwalo la milandu komwe akayankhe milandu yoitanira galimoto zomwe ndi zosemphana ndi malamulo
Female
Pamenepa, mneneri wa polisi ya Blantyreyu wachenjeza anyamata ena omwe amachita izi mu mzindawu kuti nawonso akapezeka amangidwa
Pamenepa, mneneri wa polisi ya Bulantaya yu wachenjeza anyamata ena omwe amachita izi mu mzindawu kuti nawonso akapezeka amangidwa
Female
Izitu zikuza ngakhale pali mtsutso waukulu pakati pa anthu, ngati ndi koyenera kuti boma lichotse anyamatawa m’malo omwe amakhala akuitanira galimoto maka polingaliranso mavuto a zachuma omwe akuta anthu m’dziko muno
Izitu zikuza ngakhale pali mtsutso waukulu pakati pa anthu, ngati ndi koyenera kuti boma lichotse anyamatawa m’malo omwe amakhala akuitanira galimoto maka polingaliranso mavuto a zachuma omwe akuta anthu m’dziko muno
Female
Boma lakana pempho la bungwe la eni minibus mdziko muno la Minibus Owners Association of Malawi (MOAM)
Boma lakana pempho la bungwe la eni minibasi mdziko muno la Minibasi onazi asosiyeshoni ofu Malawi (mowamu)
Female
loti mitengo ya ndalama zomwe ma minibus wa azipereka akamadutsa pa zipata za Chingeni ku Ntcheu ndi Kalinyeke ku Dedza, aitsitse
loti mitengo ya ndalama zomwe ma minibasi wa azipereka akamadutsa pa zipata za Chingeni ku Ntcheu ndi Kalinyeke ku Dedza, aitsitse
Female
Boma kudzera mwa mneneri wake, Gospel Kazako lauza olemba nkhani mu mzinda wa wa Blantyre kuti mitengo yomwe boma linaika ndi yotsika kwambiri poyerekeza ndi maiko ena a mdera la ku chigwa kwa Africa
Boma kudzera mwa mneneri wake, Gosipelo Kazako lauza olemba nkhani mu mzinda wa wa Bulantaya kuti mitengo yomwe boma linaika ndi yotsika kwambiri poyerekeza ndi maiko ena a mdera la ku chigwa kwa Afilika
Female
Mau a Kazako adza pomwe eni ma minibus wa aopseza kuti kuyambira mawa lolemba ayambe kunyanyala ntchito pofuna kuumiliza bomali kuti limve Pempho lawo pa nkhaniyi
Mau a Kazako adza pomwe eni ma minibasi wa aopseza kuti kuyambira mawa lolemba ayambe kunyanyala ntchito pofuna kuumiliza bomali kuti limve Pempho lawo pa nkhaniyi
Female
Apa a Kazako ati m’zika iliyonse ili ndi ufulu ochita zionetsero ndipo boma silikutekeseka ndi ganizo lonyanyala ntchitoli
Apa a Kazako ati m’zika iliyonse ili ndi ufulu ochita zionetsero ndipo boma silikutekeseka ndi ganizo lonyanyala ntchitoli
Female
Bungwe la boma la Roads Fund Administration (RFA) linakhazikitsa mtengo wa K3,400 kuti ndi omwe minibus zizilipira nthawi iliyonse zikudutsa pa zipatazi
Bungwe la boma la lodzi fandi adiminisitileshoni (ala efue) linakhazikitsa mtengo wa fili sauzande folo handiledi kwacha kuti ndi omwe minibasi zizilipira nthawi iliyonse zikudutsa pa zipatazi
Female
mtengo omwe malingana ndi MOAM ndi okwera kwambiri ndipo akuti ukuyenera kutsika mpaka pa K500
mtengo omwe malingana ndi mowamu ndi okwera kwambiri ndipo akuti ukuyenera kutsika mpaka pa faifi handiledi kwacha
Female
Boma lachenjeza kuthana ndi mafumu ena omwe a mtundu wa a Chewa omwe akukonza zokachita m’bindikiro ku ofesi ya mtsogoleri wa dziko lino ati ndi cholinga chofuna kukamiza president-yu kuti awakweze
Boma lachenjeza kuthana ndi mafumu ena omwe a mtundu wa a Chewa omwe akukonza zokachita m’bindikiro ku ofesi ya mtsogoleri wa dziko lino ati ndi cholinga chofuna kukamiza pulezidenti yu kuti awakweze
Female
Mafumuwa omwe ndi ochokera m’maboma a Dowa ndi Ntchitsi akuti akufuna mtsogoleriyu awakweze kuchoka pa udindo wa mfumu ya m’mudzi ndi kukakhala mafumu aakulu
Mafumuwa omwe ndi ochokera m’maboma a Dowa ndi Ntchitsi akuti akufuna mtsogoleriyu awakweze kuchoka pa udindo wa mfumu ya m’mudzi ndi kukakhala mafumu aakulu
Female
Komatu wachiwiri
Komatu wachiwiri
Female
ndipo anaonjezera kuti izi zili ndi kuthekera kosokoneza chitetezo komanso mtendere ku ofesi ya mtsogoleri
ndipo anaonjezera kuti izi zili ndi kuthekera kosokoneza chitetezo komanso mtendere ku ofesi ya mtsogoleri
Female
Wachiwiri kwa Ndunayi yadzudzulanso bungwe la Bwalo la Achewa Foundation ponena kuti ndi lomwe likutsogoleri kuti mafumuwa achite za upanduzi
Wachiwiri kwa Ndunayi yadzudzulanso bungwe la Bwalo la Achewa Faundeshoni ponena kuti ndi lomwe likutsogoleri kuti mafumuwa achite za upanduzi
Female
Pakadali pano, a Daudi ati kukweza mafumu kamachitika m’madera omwe mafumuwa amachokera osati boma. Kwa Jenda M’boma la Mzimba, mnyamata wazaka 16 ali m’chitokosi cha apolisi
Pakadali pano, a Daudi ati kukweza mafumu kamachitika m’madera omwe mafumuwa amachokera osati boma. Kwa Jenda M’boma la Mzimba, mnyamata wazaka sikisitini ali m’chitokosi cha apolisi
Female
pomuganizira kuti wagwilira mwana wazaka 13 zakubadwa. Mneneri wa polisi ya Jenda, Martha Msamali, watsimikiza za kumangidwa kwa mnyamatayu
pomuganizira kuti wagwilira mwana wazaka fetini zakubadwa. Mneneri wa polisi ya Jenda, Mafa Msamali, watsimikiza za kumangidwa kwa mnyamatayu
Female
yemwe ndi ophunzira wa Form 1 pa sukulu yoyendera ya Ehesheni CDSS. Oganiziridwa-yu ndi wa m’mudzi mwa Zamani m’dera la mfumu yaikulu Mzikowola m’boma la Mzimba
yemwe ndi ophunzira wa fomu wani pa sukulu yoyendera ya Ehesheni sidiesiesi. Oganiziridwa-yu ndi wa m’mudzi mwa Zamani m’dera la mfumu yaikulu Mzikowola m’boma la Mzimba
Female
ndipo akawonekera mu bwalo la Milandu posachedwapa. Nthambi yowona za anthu olowa komanso kutuluka m'dziko latumiza kwawo nzika ziwiri za m'dziko la Tanzania
ndipo akawonekera mu bwalo la Milandu posachedwapa. Nthambi yowona za anthu olowa komanso kutuluka m'dziko latumiza kwawo nzika ziwiri za m'dziko la Tanzaniya
Female
kaamba kopezeka zikukhala m'dziko muno opanda kalata zowayeneleza. Mneneri ku nthambiyi, Wellington Chiponde, watsimikiza za nkhaniyi pomwe wati awiriwa ndi a Jastine Kashum komanso Stephano Karura
kaamba kopezeka zikukhala m'dziko muno opanda kalata zowayeneleza. Mneneri ku nthambiyi, Weling’itoni Chiponde, watsimikiza za nkhaniyi pomwe wati awiriwa ndi a Jasitini Kashumu komanso Sitefano Karura
Female
Malingana ndi a Chiponde, awiriwa anamangidwa pa 27 mwezi uno mu mzinda wa Blantyre
Malingana ndi a Chiponde, awiriwa anamangidwa pa twente seveni mwezi uno mu mzinda wa Bulantaya
Female
Anthu omwe sakudziwika akhapa gavanala wa chipani cha DPP ku chigawo cha ku m'mwera a Charles Mchacha
Anthu omwe sakudziwika akhapa gavanala wa chipani cha Dipipi ku chigawo cha ku m'mwera a Tchalosi Mchacha
Female
A Mchacha poyankhula ndi nyumba ina yofalitsa nkhani m'dziko muno ati anthu-wa omwe analipo pafupifupi khumi ndi asanu awachita chipongwechi ku nyumba kwawo ya kwa Bvumbwe
A Mchacha poyankhula ndi nyumba ina yofalitsa nkhani m'dziko muno ati anthuwa omwe analipo pafupifupi khumi ndi asanu awachita chipongwechi ku nyumba kwawo ya kwa Bvumbwe
Female
Malipoti akuti pakadali pano a Mchacha agonekedwa ku chipatala cha Queen Elizabeth Central mu mzinda wa Blantyre komwe akulandira thandizo la mankhwala
Malipoti akuti pakadali pano a Mchacha agonekedwa ku chipatala cha Kwini elizabefi sentilo mu mzinda wa Bulantaya komwe akulandira thandizo la mankhwala
Female
Bambo wa zaka 36, Joseph Ntonya yemwe amayendetsa galimoto ya matola mu mzinda wa Blantyre ali mchitokosi cha apolisi pomuganizira kuti wagwililira kasitomala wake
Bambo wa zaka fete sikisi, Jozefe Ntonya yemwe amayendetsa galimoto ya matola mu mzinda wa Bulantaya ali mchitokosi cha apolisi pomuganizira kuti wagwililira kasitomala wake
Female
Mneneri wa polisi ya Blantyre, Peter Mchiza watiuza kuti apolisi akuganizila kuti mkuluyu anapalamula mlanduwu usiku wa pa 16 October chaka chino pa tchalitchi cha Winners Chapel ku Chitawira mu mzindawu
Mneneri wa polisi ya Blantaya, Pita Mchiza watiuza kuti apolisi akuganizila kuti mkuluyu anapalamula mlanduwu usiku wa pa sikisitini Okutoba chaka chino pa tchalitchi cha winazi tchapelo ku Chitawira mu mzindawu
Female
Nkhaniyi ikuti kasitomalayu anali pa malo omwera mowa a Blue Elephant ndipo kaamba koledzera kwambiri, anapanga hayala galimoto yomwe nambala yake ndi CK 7495 yomwe imayendetsedwa ndi oganizilidwayu
Nkhaniyi ikuti kasitomalayu anali pa malo omwera mowa a Bulu elefanti ndipo kaamba koledzera kwambiri, anapanga hayala galimoto yomwe nambala yake ndisikeyi sevente folo nainte faifi yomwe imayendetsedwa ndi oganizilidwayu
Female
Malingana ndi malipoti a apolisi, ali mu njira kulunjika ku nyumba ya maiyu, Ntonya anaima pa tchalitchi cha Winners Chapel ndi kumugwililira koma maiyu osazindikira kalikonse kaamba koti anali ataledzera kwambiri
Malingana ndi malipoti a apolisi, ali mu njira kulunjika ku nyumba ya maiyu, Ntonya anaima pa tchalitchi cha Winazi tchapelo ndi kumugwililira koma maiyu osazindikira kalikonse kaamba koti anali ataledzera kwambiri
Female
Ndipo atazindikira kuti wachitidwa chiponwechi, ndi pomwe amakaitula nkhaniyi m’manja mwa apolisi omwe sanachedwe koma kumanga Ntonya ndipo akuti amutengera ku bwalo la milandu posachedwapa komwe akayankhe mlandu ogwililira
Ndipo atazindikira kuti wachitidwa chiponwechi, ndi pomwe amakaitula nkhaniyi m’manja mwa apolisi omwe sanachedwe koma kumanga Ntonya ndipo akuti amutengera ku bwalo la milandu posachedwapa komwe akayankhe mlandu ogwililira
Female
Josepha Ntonya ndi wa m’mudzi mwa Mpagaja mfumu yaikulu Somba ku Blantyre
Josefa Ntonya ndi wa m’mudzi mwa Mpagaja mfumu yaikulu Somba ku Blantyre
Female
Madera ena a mu mzinda wa Blantyre kukugwa Mvula usiku uno. Tatiuzeni momwe yengo iliri kwanuko kudzera mu bokosi la ndemanga m'musimu
Madera ena a mu mzinda wa Bulantaya kukugwa Mvula usiku uno. Tatiuzeni momwe yengo iliri kwanuko kudzera mu bokosi la ndemanga m'musimu
Female
Polisi ya Nkhunga m'boma la Nkhotakota yatsekera mchitokosi amuna anayi powaganizira kuti anaba njinga ya moto ya kampani yopanga sugar ya Illovo
Polisi ya Nkhunga m'boma la Nkhotakota yatsekera mchitokosi amuna anayi powaganizira kuti anaba njinga ya moto ya kampani yopanga shuga ya Ilovo
Female
Ofalitsa nkhani za polisi ya Nkhunga, Thandiwe Maseko watiuza kuti amunawa ndi a Ganizani Medson, a Havila Maxwell, a Sangalalani Brown
Ofalitsa nkhani za polisi ya Nkhunga, Thandiwe Maseko watiuza kuti amunawa ndi a Ganizani Medisoni, a Havila Makisiwelo, a Sangalalani Bulauni
Female
a m’mudzi mwa mfumu yaikulu Malemia ku Nsanje komanso a Kelvin Benson a m’mudzi mwa mfumu yaikulu Makwangwala ku Ntcheu
a m’mudzi mwa mfumu yaikulu Malemia ku Nsanje komanso a Keuvini Benisoni a m’mudzi mwa mfumu yaikulu Makwangwala ku Ntcheu
Female
Malingana ndi Maseko, m’modzi mwa ogwira ntchito ku kampani ya Illovo anatenga njingayi kupita nawo kwawo komwe anakaisiya pa khonde iye ndi kumagona, koma potuluka panja anapeza kuti palibe
Malingana ndi Maseko, m’modzi mwa ogwira ntchito ku kampani ya Ilovo anatenga njingayi kupita nawo kwawo komwe anakaisiya pa khonde iye ndi kumagona, koma potuluka panja anapeza kuti palibe
Female
Apa nkhaniyi anakaitula ku polisi ndipo kafuku-fuku anayambika zomwe zachititsa kuti amunawa amangidwe
Apa nkhaniyi anakaitula ku polisi ndipo kafuku-fuku anayambika zomwe zachititsa kuti amunawa amangidwe
Female
Mneneri wa polisi ya Nkhunga-yi wati anthu-wa akaonekera ku bwalo la milandu posachedwapa kukayankha mlandu okuba
Mneneri wa polisi ya Nkhunga-yi wati anthu-wa akaonekera ku bwalo la milandu posachedwapa kukayankha mlandu okuba
Female
Banja lina ku Ndirande-Majiga mu mzinda wa Blantyre lakunthana modetsa nkhawa kaamba ka kuti bambo wa mnyumbayi anagula nsalu imodzi ya anakubala yomwe anakapereka kwa mayi ake okha
Banja lina ku Ndirande-Majiga mu mzinda wa Bulantaya lakunthana modetsa nkhawa kaamba ka kuti bambo wa mnyumbayi anagula nsalu imodzi ya anakubala yomwe anakapereka kwa mayi ake okha
Female
Nkhaniyi ikuti bamboyu anagula nsaluyo ndipo anakayipereka kwa mayi ake ngati mphatso ya anakubala
Nkhaniyi ikuti bamboyu anagula nsaluyo ndipo anakayipereka kwa mayi ake ngati mphatso ya anakubala
Female
koma izi sizinasangalatse mkazi wake ponena kuti naye akufuna nsalu yoti akapere kwa mayi ake. Koma atafunsa mamuna wakeyu chifukwa chimene anagulira nsalu ya mai ake okha mamunayu anayakha m’maso muli gwaa
koma izi sizinasangalatse mkazi wake ponena kuti naye akufuna nsalu yoti akapere kwa mayi ake. Koma atafunsa mamuna wakeyu chifukwa chimene anagulira nsalu ya mai ake okha mamunayu anayakha m’maso muli gwaa
Female
kuti tsiku la anakubala limatathauza kuti aliyese awonetse chikondi kwa amayi ake omubereka. Bamboyu anapitiliza kuwuza mkazi wakeyu
kuti tsiku la anakubala limatathauza kuti aliyese awonetse chikondi kwa amayi ake omubereka. Bamboyu anapitiliza kuwuza mkazi wakeyu
Female
kuti nayeso akagwire ganyu kuti apeze ndalama zogulira nsalu ya nakubala ya mayi ake yankho lomwe silinasangalatse mayiyu
kuti nayeso akagwire ganyu kuti apeze ndalama zogulira nsalu ya nakubala ya mayi ake yankho lomwe silinasangalatse mayiyu
Female
mpaka ndeu ya fumbi inabuka pakati pa awiri aku mbali inayi anthu akuwombera manja ngati akuwonelera kanema. Banjali pakadali pano likuyenda mwamanyazi kaamba koti anthu ambiri akuwaseka ponena kuti chifukwa chomwe amamenyana ndichopanda pake
mpaka ndeu ya fumbi inabuka pakati pa awiri aku mbali inayi anthu akuwombera manja ngati akuwonelera kanema. Banjali pakadali pano likuyenda mwamanyazi kaamba koti anthu ambiri akuwaseka ponena kuti chifukwa chomwe amamenyana ndichopanda pake
Female
Ena mwa Mamembala a komiti ya Public Accounts (PAC) ya ku nyumba ya malamulo apereka chidziwitso chawo kwa sipikala wa nyumbayi choti akufuna achotse wa pa mpando wawo, a Shadreck Namalomba
Ena mwa Mamembala a komiti ya pabuliki akauntsi (PAKI) ya ku nyumba ya malamulo apereka chidziwitso chawo kwa sipikala wa nyumbayi choti akufuna achotse wa pa mpando wawo, a Shadileki Namalomba
Female
A Namalomba omwe ndi phungu wa nyumbayi komanso mneneri wa chipani chotsutsa boma cha DPP akufuna kuchotsedwa ati kaamba kosowa khalidwe komanso mwambo.Malingana ndi chidziwitsochi chomwe aphungu khumi ndi atatu
A Namalomba omwe ndi phungu wa nyumbayi komanso mneneri wa chipani chotsutsa boma cha Dipipi akufuna kuchotsedwa ati kaamba kosowa khalidwe komanso mwambo.Malingana ndi chidziwitsochi chomwe aphungu khumi ndi atatu
Female
ambiri mwa iwo kukhala a chipani cha Malawi Congress, asainira, izi ndi kutsatira kalata yomwe wa pa mpandoyu anatulutsa
ambiri mwa iwo kukhala a chipani cha Malawi kongilesi, asainira, izi ndi kutsatira kalata yomwe wa pa mpandoyu anatulutsa
Female
ngati mneneri wa chipani youza bungwe lothana ndi Katengale ndi ziphuphu la ACB kuti lisiye kuzunza mtsogoleri wakale wa dziko lino, a Peter Mutharika
ngati mneneri wa chipani youza bungwe lothana ndi Katengale ndi ziphuphu la esibi kuti lisiye kuzunza mtsogoleri wakale wa dziko lino, a Pita Mutharika
Female
M’modzi mwa membala a komitiyi, George Zulu wati uku ndi kusowa khalidwe kwakukulu choncho a Namalomba sakuyenera kukhala wa pa mpando wa PAC
M’modzi mwa membala a komitiyi, joji Zulu wati uku ndi kusowa khalidwe kwakukulu choncho a Namalomba sakuyenera kukhala wa pa mpando wa PAKI
Female
Izi zikudza, pomwe posachedwapa nalo bungwe lomenyera ufulu wa anthu la HRDC linatulutsa kalata youza a Namalomba kuti atule pansi udindo wawo pa zifukwa za ngati zomwezi Koma phungu wa DPP yu
Izi zikudza, pomwe posachedwapa nalo bungwe lomenyera ufulu wa anthu la etchi aladisi linatulutsa kalata youza a Namalomba kuti atule pansi udindo wawo pa zifukwa za ngati zomwezi Koma phungu wa Dipipi yu
Female
wakhala akunena kuti palibe cholakwika chomwe anachita chifukwa pa nthawiyi amagwira ntchito ngati mneneri wa chipani osati wa pa mpando wa PAC
wakhala akunena kuti palibe cholakwika chomwe anachita chifukwa pa nthawiyi amagwira ntchito ngati mneneri wa chipani osati wa pa mpando wa PAKI
Female
Bwalo la milandu m’boma la Salima lalamula mayi wina wazaka 66, Nelia Gomani, kukakhala ku ndende kwa zaka 4
Bwalo la milandu m’boma la Salima lalamula mayi wina wazaka sikisite sikisi, Neliya Gomani, kukakhala ku ndende kwa zaka folo
Female
kaamba kopezeka olakwa pa mlandu ogwilira mwana wazaka 17 zakubadwa m’bomali.Tiuzeni Maganizo Anu Kodi Chilango Chimenechi Ndi Chokwanira kwa mayiyu
kaamba kopezeka olakwa pa mlandu ogwilira mwana wazaka seventini zakubadwa m’bomali.Tiuzeni Maganizo Anu Kodi Chilango Chimenechi Ndi Chokwanira kwa mayiyu
Female
Bwalo la milandu m’boma la Thyolo lagamula amuna awiri kukakhala ku ndende kwa zaka 18 aliyense atapezeka olakwa pa milandu yogwilira
Bwalo la milandu m’boma la Thyolo lagamula amuna awiri kukakhala ku ndende kwa zaka eitini aliyense atapezeka olakwa pa milandu yogwilira
Female
Amunawa ndi a Patrick Makawa omwe amadziwika kuti Sister Fire komanso Patrick Basikolo ndipo onse ali ndi zaka 45
Amunawa ndi a Patiliki Makawa omwe amadziwika kuti Sisita faya komanso Patiliki Basikolo ndipo onse ali ndi zaka fote faifi
Female
Bwalolo linamva kudzera mwa yemwe amaimira boma pa mlanduwu, Ishmael Abubast kuti Sister Fire anapamula anapalamula mlanduwu m’mwezi wa March Chaka chino pamene a Basikolo anaupalamula m’mwezi wa November chaka chatha
Bwalolo linamva kudzera mwa yemwe amaimira boma pa mlanduwu, ishumaeli abubasiti kuti sisita faya anapamula anapalamula mlanduwu m’mwezi wa Machi Chaka chino pamene a Basikolo anaupalamula m’mwezi wa Novemba chaka chatha
Female
Malingana ndi Abubast, opalamula oyambayu anagwilira mwana wa zaka 12 pomwe amakatunga madzi pa mudzi wina ku Thyolo komweko
Malingana ndi Abubasiti, opalamula oyambayu anagwilira mwana wa zaka twelofu pomwe amakatunga madzi pa mudzi wina ku Thyolo komweko
Female
pamene opalamula wachiwiriyu anagwilira mwana wake wa zaka 9, yemwe ndi omupeza, pa nthawi yomwe mai ake anali kotola nkhuni
pamene opalamula wachiwiriyu anagwilira mwana wake wa zaka naini, yemwe ndi omupeza, pa nthawi yomwe mai ake anali kotola nkhuni
Female
Koma poyankhapo, Basikolo anaukana mlanduwu zomwe zinachititsa mbali ya boma kubweretsa mboni kuzatsimikizira izi pamene Sister Fire anauvomera mbali inayi akupempha bwalo kuti lisamupatse chilango chokhwima
Koma poyankhapo, Basikolo anaukana mlanduwu zomwe zinachititsa mbali ya boma kubweretsa mboni kuzatsimikizira izi pamene sisita faya anauvomera mbali inayi akupempha bwalo kuti lisamupatse chilango chokhwima
Female
ponena kuti ali ndi banja lomwe amayang’anira. Popereka chigamulo chake, Oweruza Asunta Maxwell anati khalidweli ndi lonyasa ndipo ndi koyenera kuti abambowa akakhale ku ndende pofuna kuti atengerepo phunziro
ponena kuti ali ndi banja lomwe amayang’anira. Popereka chigamulo chake, Oweruza Asunta Makisiwelo anati khalidweli ndi lonyasa ndipo ndi koyenera kuti abambowa akakhale ku ndende pofuna kuti atengerepo phunziro
Female
Sister Fire ndi a m’mudzi mwa mfumu yaikulu Chikowi m’boma la Zomba pamene Basikolo ndi wa m’mudzi mwa mfumu yaikulu Chikumbu ku Mulanje
sisita faya ndi a m’mudzi mwa mfumu yaikulu Chikowi m’boma la Zomba pamene Basikolo ndi wa m’mudzi mwa mfumu yaikulu Chikumbu ku Mulanje
Female
Mtsogoleri wakale wa dziko lino, Peter Mutharika dzulo anagwiritsa ntchito mwambo wa chikhalidwe wa Mulhakho Wa Alhomwe
Mtsogoleri wakale wa dziko lino, Pita Mutharika dzulo anagwiritsa ntchito mwambo wa chikhalidwe wa Mulakho Wa Alomwe
Female
kukumbutsa anthu otsatira chipani cha DPP kuti chipanichi chizachititsa msonkhano wake waukulu mchaka cha 2023, monga malamulo ake akunenera
kukumbutsa anthu otsatira chipani cha Dipipi kuti chipanichi chizachititsa msonkhano wake waukulu mchaka cha twente twente fili, monga malamulo ake akunenera
Female
Iwo ayankhula izi pomwe anthu ena mchipanichi aonetsa kale chidwi chofuna kutenga utsogoleri wa chipanichi omwe pakadali pano uli m’manja mwa a Mutharikawa
Iwo ayankhula izi pomwe anthu ena mchipanichi aonetsa kale chidwi chofuna kutenga utsogoleri wa chipanichi omwe pakadali pano uli m’manja mwa a Mutharikawa
Female
Mtsogoleri wa DPP-yu wati anasankhidwa mosata malamulo choncho ndi zosayenera kuti malamulowo aphwanyidwe pongofuna kusintha utsogoleri wa chipani
Mtsogoleri wa Dipipi yu wati anasankhidwa motsata malamulo choncho ndi zosayenera kuti malamulowo aphwanyidwe pongofuna kusintha utsogoleri wa chipani
Female
Kuchokera pomwe DPP inachoka m’boma chaka chatha, pakhala pali kusamvana pakati pa akulu-akulu a chipanichi maka pa nkhani ya utsogoleri ndi mfundo zina
Kuchokera pomwe Dipipi inachoka m’boma chaka chatha, pakhala pali kusamvana pakati pa akulu-akulu a chipanichi maka pa nkhani ya utsogoleri ndi mfundo zina
Female
Koma poyankhula pa mwambo wa chikhalidwe omwewu, wa pa mpando wa chipani cha UDF yemwenso ndi mtsogoleri opuma wa dziko lino, Bakili Muluzi anadzudzula zomwe zikuchitika mchipani cha DPP
Koma poyankhula pa mwambo wa chikhalidwe omwewu, wa pa mpando wa chipani cha yudiefu yemwenso ndi mtsogoleri opuma wa dziko lino, Bakili Muluzi anadzudzula zomwe zikuchitika mchipani cha Dipipi
Female
mbali inayi akuuza a Mutharika kuti apeze mayankho a izi mwachangu. M’mau ake, wa pa mpando wa bungwe la Mulhakho Wa Alhomwe, a Leston Muli anati bungweli limakonda chikhalidwe
mbali inayi akuuza a Mutharika kuti apeze mayankho a izi mwachangu. M’mau ake, wa pa mpando wa bungwe la Mulakho Wa Alomwe, a Lesitoni Muli anati bungweli limakonda chikhalidwe
Female
ndipo ichi ndi chifukwa chake anachita chothekera kuti mwambowu uchitike. Achinyamata m’dziko muno akuti ali ndi kuthekera kothandizapo pa ntchito zosiyanasiyana zomwe ndi zopindulira anthu
ndipo ichi ndi chifukwa chake anachita chothekera kuti mwambowu uchitike. Achinyamata m’dziko muno akuti ali ndi kuthekera kothandizapo pa ntchito zosiyanasiyana zomwe ndi zopindulira anthu
Female
posadalira boma kapena mabungwe okha. Izitu ndi malingana ndi bungwe la achinyamata la Youth Mindset Change (YMC)
posadalira boma kapena mabungwe okha. Izitu ndi malingana ndi bungwe la achinyamata la yufi maindiseti chenji (wayiemusi)
Female
lomwe kumathero a sabatayi motsogozedwa ndi atsogoleri ake anakachita ntchito za Chifundo komanso kupereka zinthu zina zothandizira kulimbikitsa ukhondo pa chipatala chachikulu cha boma la Mulanje
lomwe kumathero a sabatayi motsogozedwa ndi atsogoleri ake anakachita ntchito za Chifundo komanso kupereka zinthu zina zothandizira kulimbikitsa ukhondo pa chipatala chachikulu cha boma la Mulanje
Female
Poyankhula pambuyo popereka katunduyu komanso kuchita ntchito za Chifundozi, m’modzi wa mamembala a YMC, Rita Chitanda anati ngati achinyamata anachiona cha mnzeru kuti athandizepo
Poyankhula pambuyo popereka katunduyu komanso kuchita ntchito za Chifundozi, m’modzi wa mamembala a wayiemusi, Rita Chitanda anati ngati achinyamata anachiona cha mnzeru kuti athandizepo
Female
polingalira kuti malo ngati chipatala amafunika ukhondo okwanira. Naye Chimwemwe Malibwana yemwenso ndi membala wa Youth Mindset Change (YMC) anadzudzula achinyamata amnzake
polingalira kuti malo ngati chipatala amafunika ukhondo okwanira. Naye Chimwemwe Malibwana yemwenso ndi membala wa yufi maindiseti chenji (wayiemusi) anadzudzula achinyamata amnzake
Female
omwe saonetsa chidwi pofuna kothandizapo pa ntchito zosiyanasiyana zopindulira anthu m’dziko muno. Ngati achinyamata titachilimika kumatengapo gawo ndi kuthandiza pa zinthu zina
omwe saonetsa chidwi pofuna kothandizapo pa ntchito zosiyanasiyana zopindulira anthu m’dziko muno. Ngati achinyamata titachilimika kumatengapo gawo ndi kuthandiza pa zinthu zina
Female
dziko lathu litha kutukuka mosavuta, anatero Malibwana. Mwa zina, gulu la YMC lapereka thandizo la zipangizo zotailamo zinyalala, mabigili osambira m’manja komanso kukolopera
dziko lathu litha kutukuka mosavuta, anatero Malibwana. Mwa zina, gulu la wayiemusi lapereka thandizo la zipangizo zotailamo zinyalala, mabigili osambira m’manja komanso kukolopera
Female
masache komanso katundu wina yemwe ndi wa ndalama zopitilira K500,000. zomwe achinyamatawa anachita kusonkha
masache komanso katundu wina yemwe ndi wa ndalama zopitilira faifi handiledi sauzande kwacha zomwe achinyamatawa anachita kusonkha
Female
Gulu la YMC lomwe linayambira pa tsamba la mchezo la WhatsApp akuti pakadali pano liri ndi nthambi zake m’dziko lonse la Malawi
Gulu la wayiemusi lomwe linayambira pa tsamba la mchezo la watsapu akuti pakadali pano liri ndi nthambi zake m’dziko lonse la Malawi
Female
Achinyamata m’dziko muno akuti ali ndi kuthekera kothandizapo pa ntchito zosiyanasiyana zomwe ndi zopindulira anthu posadalira boma kapena mabungwe okha
Achinyamata m’dziko muno akuti ali ndi kuthekera kothandizapo pa ntchito zosiyanasiyana zomwe ndi zopindulira anthu posadalira boma kapena mabungwe okha
Female
Izitu ndi malingana ndi bungwe la achinyamata la Youth Mindset Change (YMC) lomwe kumathero a sabatayi
Izitu ndi malingana ndi bungwe la achinyamata la yufi maindiseti chenji (wayiemusi) lomwe kumathero a sabatayi
Female
motsogozedwa ndi atsogoleri ake anakachita ntchito za Chifundo komanso kupereka zinthu zina zothandizira kulimbikitsa ukhondo pa chipatala chachikulu cha boma la Mulanje
motsogozedwa ndi atsogoleri ake anakachita ntchito za Chifundo komanso kupereka zinthu zina zothandizira kulimbikitsa ukhondo pa chipatala chachikulu cha boma la Mulanje
Female
Poyankhula pambuyo popereka katunduyu komanso kuchita ntchito za Chifundozi, m’modzi wa mamembala a YMC, Rita Chitanda
Poyankhula pambuyo popereka katunduyu komanso kuchita ntchito za Chifundozi, m’modzi wa mamembala a wayiemusi, Rita Chitanda
Female
anati ngati achinyamata anachiona cha mnzeru kuti athandizepo polingalira kuti malo ngati chipatala amafunika ukhondo okwanira
anati ngati achinyamata anachiona cha mnzeru kuti athandizepo polingalira kuti malo ngati chipatala amafunika ukhondo okwanira
Female
Bwalo la Milandu mu mzinda wa Blantyre lalamula mpondamatiki Thomson Mpinganjira kukakhala kundende kwa zaka 9 kutsatira kupezeka kwake olakwa pa mlandu ofuna kupereka ziphuphu kwa Oweruza milandu
Bwalo la Milandu mu mzinda wa Bulantaya lalamula mpondamatiki Thomusoni Mpinganjira kukakhala kundende kwa zaka naini kutsatira kupezeka kwake olakwa pa mlandu ofuna kupereka ziphuphu kwa Oweruza milandu
Female
Oweruza mlandu Dorothy DeGabrielle ndi yemwe wapereka chigamulochi lero pomwe wati mlandu omwe anapalamula a Mpinganjira ndi unali wa ukulu kwambiri chomcho akuyenera kukakhala ku ndende
Oweruza mlandu dolofe DeGabuliele ndi yemwe wapereka chigamulochi lero pomwe wati mlandu omwe anapalamula a Mpinganjira ndi unali wa ukulu kwambiri chomcho akuyenera kukakhala ku ndende
Female
A Mpinganjira ati ankafuna kupereka ziphuphu kwa Oweruza asanu omwe akaweruza mlandu okhuza chisankho cha mtsogoleri wa dziko chomwe chinachitika m’chamu 2019
A Mpinganjira ati ankafuna kupereka ziphuphu kwa Oweruza asanu omwe akaweruza mlandu okhuza chisankho cha mtsogoleri wa dziko chomwe chinachitika m’chamu twente naintini
Female
Malingana umboni omwe unaperekedwa ku bwalo la Milandu, a Mpinganjira amafuna Oweruza-wa agamule mlanduwu mokomera chipani cha Democratic Progressive , komanso a Peter Mutharika
Malingana umboni omwe unaperekedwa ku bwalo la Milandu, a Mpinganjira amafuna Oweruza-wa agamule mlanduwu mokomera chipani cha demokilatiki pulogilesivi , komanso a Pita Mutharika
Female
Bungwe la chikhalidwe la Mulhakho Wa Alhomwe lati lachinayi sabata ino likhala likupereka nsembe kwa mizimu ya makolo kuti iwathandize pa mavuto omwe akukumana nayo pakadali pano
Bungwe la chikhalidwe la Mulakho Wa Alomwe lati lachinayi sabata ino likhala likupereka nsembe kwa mizimu ya makolo kuti iwathandize pa mavuto omwe akukumana nayo pakadali pano
Female
kutsatira kusintha kwa ulamuliro kuchokera ku chipani cha DPP kupita ku chipani cha MCP
kutsatira kusintha kwa ulamuliro kuchokera ku chipani cha Dipipi kupita ku chipani cha emusipi
Female
Mkulu wa bungweli, Leston Mulli ndi yemwe wanena izi pa msonkhano wa olemba nkhani omwe unachitikira ku likulu kwa bungweli kwa Chonde m’boma la Mulanje
Mkulu wa bungweli, Lesitoni Muli ndi yemwe wanena izi pa msonkhano wa olemba nkhani omwe unachitikira ku likulu kwa bungweli kwa Chonde m’boma la Mulanje
Female
A Lhomwe m’dziko muno akukumana ndi khaza zosiyana-siyana kuchokera ku boma la Tonse chomcho ndikuyenera kupepha kwa mizimu ya makolo awo awapulumutse ku zowawazi, anatero a Mulli
A Lomwe m’dziko muno akukumana ndi khaza zosiyanasiyana kuchokera ku boma la Tonse chomcho ndikuyenera kupepha kwa mizimu ya makolo awo awapulumutse ku zowawazi, anatero a Muli
Female
Mwa zina bambo Mulli ati boma la Tonse likugwiritsa ntchito apolisi komanso bungwe lothana ndi ziphuphu la ACB pofuna kudzudza a Lhomwe m’dziko muno
Mwa zina bambo Muli ati boma la Tonse likugwiritsa ntchito apolisi komanso bungwe lothana ndi ziphuphu la esibi pofuna kudzudza a Lomwe m’dziko muno
Female