audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
Wachiwiri kwa nduna ya za chitetezo a Jean Sendeza alangiza anthu otsatira chipani cha Malawi Congress (MCP) kuti asalole anthu ena azinyoza mtsogoleri wa Chipanichi
Wachiwiri kwa nduna ya za chitetezo a Jini Sendeza alangiza anthu otsatira chipani cha Malawi kongilesi (emusipi) kuti asalole anthu ena azinyoza mtsogoleri wa Chipanichi
Female
yemwenso ndi mtsogoleri wa dziko lino, a Lazarus Chakwera. Malingana ndi malipoti a pa tsamba la mchezo la kanema wa Rainbow, -Rainbow Television Malawi
yemwenso ndi mtsogoleri wa dziko lino, a Lazalasi Chakwera. Malingana ndi malipoti a pa tsamba la mchezo la kanema wa Renibo, -Renibo Televizyoni Malawi
Female
a Sendeza ayankhula izi pa msonkhano wa ndale omwe akulu-akulu a Chipanichi anachititsa mu mzinda wa Lilongwe dzulo loweluka
a Sendeza ayankhula izi pa msonkhano wa ndale omwe akulu-akulu a Chipanichi anachititsa mu mzinda wa Lilongwe dzulo loweluka
Female
Pa msonkhanowu, nduna ya za malonda a Sosten Gwengwe ati Mavuto a za chuma omwe adza m’dziko muno ndi kaamba ka mliri wa COVID-19
Pa msonkhanowu, nduna ya za malonda a Sositeni Gwengwe ati Mavuto a za chuma omwe adza m’dziko muno ndi kaamba ka mliri wa Kovidi-naintini
Female
Ndipo m’mawu ake, mtsogoleri wa a chinyamata ku MCP a Richard Chimwendo Banda auza alangiza achinyamata otsatira Chipanichi
Ndipo m’mawu ake, mtsogoleri wa a chinyamata ku emusipi a Ritchadi Chimwendo Banda auza alangiza achinyamata otsatira Chipanichi
Female
kuti asamachitire za mtopola anthu ndi mabungwe omwe azichititsa zionetsero zosonyeza kusakondwa ndi boma la mgwirizano wa Tonse. Anthu ochuluka anasonkhana pa msonkhanowu omwe unachitikira pa bwalo la Masintha

Chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP) chauza mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera kuti atule pansi udindo
Chipani chotsutsa boma cha demokilatiki pulogilesivi (Dipipi) chauza mtsogoleri wa dziko lino, Dokota Lazalasi Chakwera kuti atule pansi udindo
Female
ponena kuti boma la mgwirizano wa Tonse lalephera kusintha zinthu m’dziko muno monga linalonjezera
ponena kuti boma la mgwirizano wa Tonse lalephera kusintha zinthu m’dziko muno monga linalonjezera
Female
Chipanichi chayankhula izi pa msonkhano wa atolankhani omwe chinachititsa mu mzinda wa Blantyre komwenso chadzudzula kolimba bomali ponena kuti lasiya njira ya chitukuko
Chipanichi chayankhula izi pa msonkhano wa atolankhani omwe chinachititsa mu mzinda wa Bulantaya komwenso chadzudzula kolimba bomali ponena kuti lasiya njira ya chitukuko
Female
ndipo tsopano likufuna kuthana ndi adani ake pa ndale. Mtsogoleri wa Chipanichi a Peter Mutharika poyankhula poyambilira pa msonkhanowu
ndipo tsopano likufuna kuthana ndi adani ake pa ndale. Mtsogoleri wa Chipanichi a Pita Mutharika poyankhula poyambilira pa msonkhanowu
Female
anati kumangidwa kwa ena mwa mamembala ake pa nkhani zomwe akuti sizoona, ndi chitsimikizo choti boma la a Chakwera likungofuna kuthana nawo chabe
anati kumangidwa kwa ena mwa mamembala ake pa nkhani zomwe akuti sizoona, ndi chitsimikizo choti boma la a Chakwera likungofuna kuthana nawo chabe
Female
Iwo adzudzula bombali kaamba kolephera kupeza mayankho pa Mavuto a za chuma omwe akuta miyoyo ya amalawi komanso tsankho lomwe akuti likuoneka kwambiri pa kasankhidwe ka maudindo m’boma
Iwo adzudzula bombali kaamba kolephera kupeza mayankho pa Mavuto a za chuma omwe akuta miyoyo ya amalawi komanso tsankho lomwe akuti likuoneka kwambiri pa kasankhidwe ka maudindo m’boma
Female
Ndipo m’mawu ake, mneneri wa Chipanichi, a Shadreck Namalomba anati boma likugwiritsa ntchito bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu la ACB komanso apolisi
Ndipo m’mawu ake, mneneri wa Chipanichi, a Shadileki Namalomba anati boma likugwiritsa ntchito bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu la esibi komanso apolisi
Female
pofuna kukhazika chete anthu omwe akulidzudzula. Apa a Namalomba auza ACB kuti isiye kukondera
pofuna kukhazika chete anthu omwe akulidzudzula. Apa a Namalomba auza esibi kuti isiye kukondera
Female
ikafuna kuchita kafuku-fuku pa nkhani zokhuza katangale pomwe auzanso bungweli kuti lifufuze momwe boma linagulitsira ndege mu ulamuliro wa chipani cha Peoples (PP)
ikafuna kuchita kafuku-fuku pa nkhani zokhuza katangale pomwe auzanso bungweli kuti lifufuze momwe boma linagulitsira ndege mu ulamuliro wa chipani cha Pipozi (PiPi)
Female
Pa msonkhanowu panalinso akulu-akulu ena a DPP monga a Joseph Mwanamveka, a Francis Mphepo komanso a Charles Mchacha
Pa msonkhanowu panalinso akulu-akulu ena a Dipipi monga a Jozefe Mwanamveka, a Fulansisi Mphepo komanso a tchalosi Mchacha
Female
omwe onse mu zoyankhula zawo, zinalunjika kwambiri pa zofooka zomwe akuti zikuoneka m’boma la Tonse
omwe onse mu zoyankhula zawo, zinalunjika kwambiri pa zofooka zomwe akuti zikuoneka m’boma la Tonse
Female
Pakadali pano, mneneri wa boma, a Gospel Kazako ati sangayankhepo kanthu pa zomwe DPP yayankhula ponena kuti sanatsatire bwino msonkhanowu
Pakadali pano, mneneri wa boma, a Gosipelo Kazako ati sangayankhepo kanthu pa zomwe Dipipi yayankhula ponena kuti sanatsatire bwino msonkhanowu
Female
Iwo auza Ndirande FM kuti ayankhe bwino akapeza tsatane-tsatane wa zomwe zayankhulidwa pa msonkhano wa atolankhaniwu
Iwo auza Ndirande efuemu kuti ayankhe bwino akapeza tsatane-tsatane wa zomwe zayankhulidwa pa msonkhano wa atolankhaniwu
Female
Ndikufuna ndimve kaye bwinobwino zomwe zayankhulidwa ndipo sikuti ndingadlire zomwe mukufotokozazi, Ndiyankha ndikapeza tsatane-tsatane, atero a Kazako
Ndikufuna ndimve kaye bwinobwino zomwe zayankhulidwa ndipo sikuti ndingadlire zomwe mukufotokozazi, Ndiyankha ndikapeza tsatane-tsatane, atero a Kazako
Female
Zionetsero zosakondwa ndi momwe boma la mgwirizano wa Tonse likuyendetsera dziko lino zayambika mu mzinda wa Lilongwe
Zionetsero zosakondwa ndi momwe boma la mgwirizano wa Tonse likuyendetsera dziko lino zayambika mu mzinda wa Lilongwe
Female
Poyamba pa zionetserozi, apolisi athira utsi okhetsa msonzi pofuna kuletsa anthu ena omwe amafuna kugwiritsa ntchito njira yosiyana
Poyamba pa zionetserozi, apolisi athira utsi okhetsa msonzi pofuna kuletsa anthu ena omwe amafuna kugwiritsa ntchito njira yosiyana
Female
ndi yomwe achitetezo-wa agwirizana ndi atsogoleri a zionetserozi kuti agwiritse ntchito
ndi yomwe achitetezo-wa agwirizana ndi atsogoleri a zionetserozi kuti agwiritse ntchito
Female
Anthu ochuluka akutenga nawo mbali pa zionetserozi ndipo pali chiyembekezo choti akasiya kalata ya madandaulo awo ku ofesi ya bwanamkubwa wa Lilongwe
Anthu ochuluka akutenga nawo mbali pa zionetserozi ndipo pali chiyembekezo choti akasiya kalata ya madandaulo awo ku ofesi ya bwanamkubwa wa Lilongwe
Female
Bwalo la milandu la za malamulo mu mzinda wa Blantyre, lero ku m'mawaku likuyembekezeleka kupereka chigamulo chake
Bwalo la milandu la za malamulo mu mzinda wa Bulantaya, lero ku m'mawaku likuyembekezeleka kupereka chigamulo chake
Female
ngati ndi koyenera kuti lipitilire kumva mlandu wa chisankho cha mtsogoleri cha Chaka chatha omwe chipani cha DPP chinakasuma
ngati ndi koyenera kuti lipitilire kumva mlandu wa chisankho cha mtsogoleri cha Chaka chatha omwe chipani cha Dipipi chinakasuma
Female
Oweluza asanu omwe akumva nkhaniyi apeleka chigamulochi, mlangizi wa boma pa za malamulo, Thabo Chakaka Nyirenda atapempha bwalo kuti nkhaniyi ingothetsedwa, pempho lomwe ma lawyer a DPP anatsutsana nalo
Oweluza asanu omwe akumva nkhaniyi apeleka chigamulochi, mlangizi wa boma pa za malamulo, Thabo Chakaka Nyirenda atapempha bwalo kuti nkhaniyi ingothetsedwa, pempho lomwe maloya a Dipipi anatsutsana nalo
Female
Chipani cha DPP chinakagwada ku bwalolo kutsatira ku chotsedwa kwa makomishonala ena omwe anayendetsa nawo chisankho cha chaka chathachi
Chipani cha Dipipi chinakagwada ku bwalolo kutsatira ku chotsedwa kwa makomishonala ena omwe anayendetsa nawo chisankho cha chaka chathachi
Female
ponena kuti analephera kuyendetsa bwino chisankho cha mu 2019 chomwe malingana ndi bwalo la milandu, chinali ndi zolakwika zambiri
ponena kuti analephera kuyendetsa bwino chisankho cha mu twente naintini chomwe malingana ndi bwalo la milandu, chinali ndi zolakwika zambiri
Female
Kupereka chigamulochi lero, kukuyembekezereka kuyamba nthawi ya 10 koloko m'mawawu
Kupereka chigamulochi lero, kukuyembekezereka kuyamba nthawi ya teni koloko m'mawawu
Female
Chipani cha Malawi Congress (MCP) chati sichikukhutira ndi momwe bungwe la zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lagawiranso madera a aphungu a ku nyumba ya malamulo komanso makhansala
Chipani cha Malawi kongilesi (emusipi) chati sichikukhutira ndi momwe bungwe la zisankho la Malawi Elekutolo komishoni (MEKI) lagawiranso madera a aphungu a ku nyumba ya malamulo komanso makhansala
Female
Mkulu owona za zisankho m'chipanichi, Elias Chakwera, ndi yemwe wanena izi dzulo pomwe bungwe la MEC limakuna ndi akulu akulu a MCP ku nyumba ya chi mfumu ya Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe
Mkulu owona za zisankho m'chipanichi, Eliyasi Chakwera, ndi yemwe wanena izi dzulo pomwe bungwe la MEKI limakuna ndi akulu akulu a emusipi ku nyumba ya chi mfumu ya Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe
Female
Malingana ndi a Chakwera, chipani cha MCP ndi chodabwa kaamba ka kuti chigawo cha ku m'mwera chili ndi madera ambiri a phungu poyerekeza ndi chigawo chapakati
Malingana ndi a Chakwera, chipani cha emusipi ndi chodabwa kaamba ka kuti chigawo cha ku m'mwera chili ndi madera ambiri a phungu poyerekeza ndi chigawo chapakati
Female
Koma poyankhapo pa nkhawazi, wa pa mpando wa bungwe la MEC, a Chifundo Kachale auza chipani cha MCP kuti apereke lipoti lofotokozera bwino madandaulo omwe amaperekawa
Koma poyankhapo pa nkhawazi, wa pa mpando wa bungwe la Meki, a Chifundo Kachale auza chipani cha emusipi kuti apereke lipoti lofotokozera bwino madandaulo omwe amaperekawa
Female
Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yakaniza a Bon Kalindo ndi gulu lawo kuchititsa zionetsero zosakondwa ndi momwe boma la mgwirizano wa Tonse likuyendetsera dziko lino, mu mzindawu lachisanu likubwerali
Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yakaniza a Boni Kalindo ndi gulu lawo kuchititsa zionetsero zosakondwa ndi momwe boma la mgwirizano wa Tonse likuyendetsera dziko lino, mu mzindawu lachisanu likubwerali
Female
A Bon Kalindo atsimikiza za nkhaniyi poyankhula ndi nyumba ina yofalitsa nkhani poonjezera kuti auzidwa ndi khonsoloyi
A Boni Kalindo atsimikiza za nkhaniyi poyankhula ndi nyumba ina yofalitsa nkhani poonjezera kuti auzidwa ndi khonsoloyi
Female
kuti pa tsikuli, apolisi adzakhala akupeleka chitetezo pa mikumano ya nthumwi za maiko a m'bungwe la SADC
kuti pa tsikuli, apolisi adzakhala akupeleka chitetezo pa mikumano ya nthumwi za maiko a m'bungwe la SADIKI
Female
Pakadali pano, a Kalindo ati atenga kale chiletso ku bwalo la milandu chotsutsana ndi zomwe khonsolo ya Lilongwe yanena ndipo mawa lachinai, bwalolo likuyembekezeleka kumva mfundo za mbali zonse ziwiri pa nkhaniyi

Mu pologalamu yathu ya Inu Mukutinji ya sabata ino, tikukamba za ndondomeko ya boma ya Chaka chino yogulitsa zipangizo za ulimi monga feteleza pa mtengo yotsika
Mu pologalamu yathu ya Inu Mukutinji ya sabata ino, tikukamba za ndondomeko ya boma ya Chaka chino yogulitsa zipangizo za ulimi monga feteleza pa mtengo yotsika
Female
Tiuzeni momwe ndondomekoyi ikuyendera kwanuko.Tiuzeni kudzera mu comment box ndipo tiwerenga kuyambira nthawi ya 5 mpaka 6 koloko madzulo ano
Tiuzeni momwe ndondomekoyi ikuyendera kwanuko.Tiuzeni kudzera mu komenti bokosi ndipo tiwerenga kuyambira nthawi ya faifi mpaka sikisi koloko madzulo ano
Female
Bungwe loyendetsa zisankho m'dziko muno la Malawi Electoral commission ( MEC) lati atolankhani Ali ndi udindo waukulu wodziwitsa anthu zakufunika kwa ntchito younikanso malire a Madera a aphungu
Bungwe loyendetsa zisankho m'dziko muno la Malawi elekitolo komishoni ( MEKI) lati atolankhani Ali ndi udindo waukulu wodziwitsa anthu zakufunika kwa ntchito younikanso malire a Madera a aphungu
Female
komanso momwe ntchitoyi ikuyendera. Komishonala wa bungweli, Dr Emmanuel Fabiano ndi yemwe wayankhula izi lero pa maphunziro a tsiku limodzi
komanso momwe ntchitoyi ikuyendera. Komishonala wa bungweli, Dokota imanuwelo Fabiyano ndi yemwe wayankhula izi lero pa maphunziro a tsiku limodzi
Female
omwe bungweli linakonzera akulu akulu a nyumba zowulutsa ndi kutsindikiza nkhani mu mzinda wa Blantyre
omwe bungweli linakonzera akulu akulu a nyumba zowulutsa ndi kutsindikiza nkhani mu mzinda wa Bulantaya
Female
Dr Fabiano anatsindika kuti bungwe la MEC likugwira ntchito younikanso malirewa motsata malamulo
Dokota Fabiyano anatsindika kuti bungwe la MEKI likugwira ntchito younikanso malirewa motsata malamulo
Female
Dziko la Malawi pakadali pano Lili ndi Madera aphungu wokwana 193 ndipo ngati maderawa aonjezeredwe afika pa 228
Dziko la Malawi pakadali pano Lili ndi Madera aphungu wokwana wani nainte fili ndipo ngati maderawa aonjezeredwe afika pa thu twente eiti
Female
Zionetsero zosonyeza kusakondwa ndi momwe boma la mgwirizano wa Tonse likuyendetsera dziko lino zachitika lero m’mizinda ya Mzuzu ndi Blantyre
Zionetsero zosonyeza kusakondwa ndi momwe boma la mgwirizano wa Tonse likuyendetsera dziko lino zachitika lero m’mizinda ya Mzuzu ndi Bulantaya
Female
ngakhale ku Blantyre kunali zosamwitsa. Ku Mzuzu, zionetserozi zachitika motsogozedwa ndi bungwe la Social Revolution Movement lomwe limatsogozedwa ndi a Phunziro Mvula
ngakhale ku Bulantaya kunali zosamwitsa. Ku Mzuzu, zionetserozi zachitika motsogozedwa ndi bungwe la sosho livolushoni muvumenti lomwe limatsogozedwa ndi a Phunziro Mvula
Female
Ngakhale pachiyambi panali kusamvana ndi a chitetezo pa nkhani za zionetserozi, Komatu zachitika mwa bata ndi mtendere
Ngakhale pachiyambi panali kusamvana ndi a chitetezo pa nkhani za zionetserozi, Komatu zachitika mwa bata ndi mtendere
Female
kufikira pomwe anthu ochita zionetserowa anakapereka kalata ya madandaulo awo ku ofesi za khonsolo ya Mzuzu
kufikira pomwe anthu ochita zionetserowa anakapereka kalata ya madandaulo awo ku ofesi za khonsolo ya Mzuzu
Female
Ndipo Ku Blantyre Zomwe zimaoneka ngati sizichitika kaamba ka kukula kwa ziwawa zochitirana pakati pa anthu ndi apolisi
Ndipo Ku Bulantaya Zomwe zimaoneka ngati sizichitika kaamba ka kukula kwa ziwawa zochitirana pakati pa anthu ndi apolisi
Female
zionetserozi zachitika ndi Pempho loti adindo achite machawi pothana ndi Mavuto omwe akuta miyoyo ya anthu
zionetserozi zachitika ndi Pempho loti adindo achite machawi pothana ndi Mavuto omwe akuta miyoyo ya anthu
Female
Yemwe anatsogolera zionetserozi, a Bon Kalindo ati ndi zomvetsa Chisoni kuti kusintha komwe anthu amafuna palibe
Yemwe anatsogolera zionetserozi, a Boni Kalindo ati ndi zomvetsa Chisoni kuti kusintha komwe anthu amafuna palibe
Female
ndipo aonjezera kuti pali anthu ena omwe amayesa-yesa kutchinjiliza mzika kuti zisachite zionetsero zoonetsera poyera Mavuto awo
ndipo aonjezera kuti pali anthu ena omwe amayesa-yesa kutchinjiliza mzika kuti zisachite zionetsero zoonetsera poyera Mavuto awo
Female
Mwa zina, a Kalindo ati amva malipoti oti anthu ena anatumidwa kuzasokoneza zionetsero za ku Blantyre, zomwe Mapeto ake zavulalitsa anthu angapo kutsatira kubuka kwa ziwawa mu mzindawu
Mwa zina, a Kalindo ati amva malipoti oti anthu ena anatumidwa kuzasokoneza zionetsero za ku Bulantaya, zomwe Mapeto ake zavulalitsa anthu angapo kutsatira kubuka kwa ziwawa mu mzindawu
Female
Apolisi anagwiritsa ntchito utsi okhetsa msozi pofuna kukhazikika bata, kutsatira kugendana miyala komwe kunabuka, kumenya anthu ongodutsa
Apolisi anagwiritsa ntchito utsi okhetsa msozi pofuna kukhazikika bata, kutsatira kugendana miyala komwe kunabuka, kumenya anthu ongodutsa
Female
komanso kutentha polisi unit ya mu mzindawu, zomwe achita ndi anthu ochita zionetserozi
komanso kutentha polisi yuniti ya mu mzindawu, zomwe achita ndi anthu ochita zionetserozi
Female
Tinayesetsa kuti tiyankhule ndi mneneri wa boma a Gospel Kazako kuti athilirepo ndemanga pa nkhanizi, koma sanayankhe lamya yawo ya m’manja titamuimbira kangapo konse
Tinayesetsa kuti tiyankhule ndi mneneri wa boma a Gosipelo Kazako kuti athilirepo ndemanga pa nkhanizi, koma sanayankhe lamya yawo ya m’manja titamuimbira kangapo konse
Female
Pomwe apolisi anauza Atolankhani kuti zionetsero za lero zalephereka ndipo agwirizana ndi a Bon Kalindo kuti zichitike tsiku lina, zapezeka kuti zionetserozi zikuchitika
Pomwe apolisi anauza Atolankhani kuti zionetsero za lero zalephereka ndipo agwirizana ndi a Boni Kalindo kuti zichitike tsiku lina, zapezeka kuti zionetserozi zikuchitika
Female
Ndirande FM inagwira mau a mneneri wa polisi ya Blantyre, Peter Mchiza yemwe anati zionetserozi sizichitika chifukwa a Kalindo amadandaula kuti chitetezo chawo sichili bwino
Ndirande efuemu inagwira mau a mneneri wa polisi ya Bulantaya, Pita Mchiza yemwe anati zionetserozi sizichitika chifukwa a Kalindo amadandaula kuti chitetezo chawo sichili bwino
Female
Komatu pano, anthu omwe akutsogozedwa ndi a Kalindo ayamba kuchita zionetsero ndipo akukasiya kalata ya madandaulo ku ofesi za khonsolo ya mzinda wa Blantyre
Komatu pano, anthu omwe akutsogozedwa ndi a Kalindo ayamba kuchita zionetsero ndipo akukasiya kalata ya madandaulo ku ofesi za khonsolo ya mzinda wa Bulantaya
Female
Ntchito za malonda zayamba kubwelera mchimake mu mzinda wa Blantyre, zitaima kwa maola angapo kaamba ka ziwawa zomwe zinabuka pakati pa anthu omwe amafuna kuchita zionetsero
Ntchito za malonda zayamba kubwelera mchimake mu mzinda wa Bulantaya, zitaima kwa maola angapo kaamba ka ziwawa zomwe zinabuka pakati pa anthu omwe amafuna kuchita zionetsero
Female
Mwa zina, anthu-wa amagendana, kumenya ndi kuthamangitsa anthu ongodutsa komanso kuyatsa matayala munsewu
Mwa zina, anthu-wa amagendana, kumenya ndi kuthamangitsa anthu ongodutsa komanso kuyatsa matayala munsewu
Female
Kwa maola opitilira atatu, apolisi akhala akuthira utsi okhetsa msonzi pofuna kubalalitsa anthu-wa omwe ambiri mwa iwo ndi achinyamata
Kwa maola opitilira atatu, apolisi akhala akuthira utsi okhetsa msonzi pofuna kubalalitsa anthu-wa omwe ambiri mwa iwo ndi achinyamata
Female
Pakadali pano, malipoti akuti zionetserozi zalepheletsedwa kutsatira nkhawa yoti chitetezo cha a Bon Kalindo omwe amayenera kuzitsogolera, sichili bwino
Pakadali pano, malipoti akuti zionetserozi zalepheletsedwa kutsatira nkhawa yoti chitetezo cha a Boni Kalindo omwe amayenera kuzitsogolera, sichili bwino
Female
Apolisi athira utsi okhetsa msonzi pofuna kubalalitsa magulu achinyamata omwe akuchitirana ziwawa patsogolo pa zionetsero zomwe a Bon Kalindo akufuna kutsogolera
Apolisi athira utsi okhetsa msonzi pofuna kubalalitsa magulu achinyamata omwe akuchitirana ziwawa patsogolo pa zionetsero zomwe a Boni Kalindo akufuna kutsogolera
Female
Maguluwa omwe malingana ndi malipoti ndi omwe akuikira kumbuyo zionetserozi komanso kutsutsana nazo, akugendana miyala komanso kuonetsana zikwanje
Maguluwa omwe malingana ndi malipoti ndi omwe akuikira kumbuyo zionetserozi komanso kutsutsana nazo, akugendana miyala komanso kuonetsana zikwanje
Female
Maguluwa akuthamangitsanso anthu ena omwe abwera kuzatenga nawo pa zionetserozi komanso ena ongodutsa
Maguluwa akuthamangitsanso anthu ena omwe abwera kuzatenga nawo pa zionetserozi komanso ena ongodutsa
Female
Kunali ziwawa mphindi zingapo zapitazo pa bwalo la milandu la Blantyre Magistrate pomwe anthu ochita zionetsero amafuna kumenya munthu wina yemwe akumuganizira kuti ali mgulu la anthu omwe akutsutsana ndi zionetsero za lero
Kunali ziwawa mphindi zingapo zapitazo pa bwalo la milandu la Bulantaya majesitileti pomwe anthu ochita zionetsero amafuna kumenya munthu wina yemwe akumuganizira kuti ali mgulu la anthu omwe akutsutsana ndi zionetsero za lero
Female
Malingana ndi zomwe Ndirande FM yaona, munthuyu anapulumutsidwa ndi munthu wina yemwe ndi wachitetezo wa padera
Malingana ndi zomwe Ndirande efuemu yaona, munthuyu anapulumutsidwa ndi munthu wina yemwe ndi wachitetezo wa padera
Female
Apolisi omwe ndi ochuluka ali kale pa malo omwe zionetserozi ziyambire koma sanachitepo kanthu pa ziwawazi
Apolisi omwe ndi ochuluka ali kale pa malo omwe zionetserozi ziyambire koma sanachitepo kanthu pa ziwawazi
Female
Anthu omwe ambiri mwa iwo ndi achinyamata akusonkhana pa bwalo la milandu la magistrate mu mzinda wa Blantyre, ndi cholinga choti atenge nawo pa zionetsero zomwe a Bon Kalindo akuyembekezereka kutsogolera lero
Anthu omwe ambiri mwa iwo ndi achinyamata akusonkhana pa bwalo la milandu la majisitiletimu mzinda wa Bulantaya, ndi cholinga choti atenge nawo pa zionetsero zomwe a Boni Kalindo akuyembekezereka kutsogolera lero
Female
Anthuwa akuti akufuna kutenga nawo mbali pa zionetserozi ngati imodzi mwa njira yosonyeza kusakondwa ndi mavuto omwe dziko lino likukumana nawo
Anthuwa akuti akufuna kutenga nawo mbali pa zionetserozi ngati imodzi mwa njira yosonyeza kusakondwa ndi mavuto omwe dziko lino likukumana nawo
Female
Apolisi ku Limbe mu mzinda wa Blantyre ati achilimika pofuna kuonetsetsa kuti anthu komanso katundu ndi otetezeka, patangopita maola ochepa
Apolisi ku Limbe mu mzinda wa Bulantaya ati achilimika pofuna kuonetsetsa kuti anthu komanso katundu ndi otetezeka, patangopita maola ochepa
Female
ziwawa zitabuka pakati pa magulu ena omwe amapezeka mu msikawu. Magulu-wa anayamba kuchitirana ziwawa kutsatira zionetsero zomwe limodzi mwa iwo limachita
ziwawa zitabuka pakati pa magulu ena omwe amapezeka mu msikawu. Magulu-wa anayamba kuchitirana ziwawa kutsatira zionetsero zomwe limodzi mwa iwo limachita
Female
ati zosonyoza kusagwirizana ndi zionetsero zomwe a Bon Kalindo akonza zosakondwa ndi momwe boma la mgwirizano wa tonse likuyendetsera dziko lino
ati zosonyoza kusagwirizana ndi zionetsero zomwe a Boni Kalindo akonza zosakondwa ndi momwe boma la mgwirizano wa tonse likuyendetsera dziko lino
Female
Ngakhale wati sangayankhule pa nkhaniyi pakadali pano, mneneri wa polisi ya Limbe, Patrick Mussa
Ngakhale wati sangayankhule pa nkhaniyi pakadali pano, mneneri wa polisi ya Limbe, Patiliki Musa
Female
wauza Ndirande FM kuti apolisi akhala akuyang’anira malo osiyana-siyana mu msikawu ndipo watinso tsopano bata labwelera
wauza Ndirande efuemu kuti apolisi akhala akuyang’anira malo osiyana-siyana mu msikawu ndipo watinso tsopano bata labwelera
Female
Pa ziwawazi zomwe Mapeto ake apolisi anagwiritsa ntchito utsi okhetsa msonzi pofuna kukhazikitsa bata, anthu ena avulala kutsatira kukhapidwa ndi zikwanje
Pa ziwawazi zomwe Mapeto ake apolisi anagwiritsa ntchito utsi okhetsa msonzi pofuna kukhazikitsa bata, anthu ena avulala kutsatira kukhapidwa ndi zikwanje
Female
Malipoti akuti limodzi mwa maguluwa limatsogozedwa ndi khansala wa ward ya Ntopwa, Isaac Jomo Osman yemwe pamodzi ndi anyamata ake amachita zionetsero zotsutsana ndi zionetsero za mawa
Malipoti akuti limodzi mwa maguluwa limatsogozedwa ndi khansala wa wadi ya Ntopwa, aizeki Jomo Osimani yemwe pamodzi ndi anyamata ake amachita zionetsero zotsutsana ndi zionetsero za mawa
Female
koma ali mkati mochita izi, anangodabwa gulu lina layamba kuwagenda, zomwe zinakhuzanso ntchito za malonda
koma ali mkati mochita izi, anangodabwa gulu lina layamba kuwagenda, zomwe zinakhuzanso ntchito za malonda
Female
Chipani cha UTM chati ndi chodabwa komanso kukhumudwa ndi ganizo la a Bon Kalindo lotuluka mchipanichi. Mneneri wa UTM, Frank Mwenefumbo
Chipani cha yutiemu chati ndi chodabwa komanso kukhumudwa ndi ganizo la a Boni Kalindo lotuluka mchipanichi. Mneneri wa yutiemu, fulanki Mwenefumbo
Female
wauza Ndirande FM mphindi zingapo zapitazo kuti kutuluka kwa a Kalindo ndi kodandaulitsa polingalira kuti iwo ndi m'modzi mwa anthu omwe anayambitsa nawo UTM zaka zingapo zapitazo
wauza Ndirande efuemu mphindi zingapo zapitazo kuti kutuluka kwa a Kalindo ndi kodandaulitsa polingalira kuti iwo ndi m'modzi mwa anthu omwe anayambitsa nawo yutiemu zaka zingapo zapitazo
Female
Komabe, a Mwenefumbo adzudzula a Kalindo kaamba kosiya katundu wa chipani pa nsewu, ponena kuti izi sizabwino chifukwa katunduyu anamutengera ku ofesi ndipo amayenera kukasiyanso ku ofesi
Komabe, a Mwenefumbo adzudzula a Kalindo kaamba kosiya katundu wa chipani pa nsewu, ponena kuti izi sizabwino chifukwa katunduyu anamutengera ku ofesi ndipo amayenera kukasiyanso ku ofesi
Female
Pomwe amalangeza kuti atuluka ku UTM ku Dorvic Hotel mu mzinda wa Blantyre, a Kalindo anauzanso atolankhani kuti galimoto ya chipani yomwe amayendera aisiya ku hotel komweko
Pomwe amalangeza kuti atuluka ku yutiemu ku Doviki Hotelo mu mzinda wa Bulantaya, a Kalindo anauzanso atolankhani kuti galimoto ya chipani yomwe amayendera aisiya ku hotelo komweko
Female
ndipo kuti akuluakulu a UTM akaitenge okha. Mkulu wa achinyamata mchipani cha UTM a Bon Kalindo lero akuchititsa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Blantyre
ndipo kuti akuluakulu a yutiemu akaitenge okha. Mkulu wa achinyamata mchipani cha yutiemu a Boni Kalindo lero akuchititsa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Bulantaya
Female
komwe mwa zina akufotokoza zambiri zokhuza zionetsero zomwe a Kalindowa akonza. A Kalindo achititsa zionetserozi m'mizinda ikulu-ikulu ya dziko lino
komwe mwa zina akufotokoza zambiri zokhuza zionetsero zomwe a Kalindowa akonza. A Kalindo achititsa zionetserozi m'mizinda ikulu-ikulu ya dziko lino
Female
ati kusonyeza kusakondwa ndi momwe utsogoleri wa boma la Tonse ukuyendetsera dziko lino. Mwa zina, iwo akudzudzula tsankho posankhana maudindo lomwe akuti lamanga nthenje m'dziko muno
ati kusonyeza kusakondwa ndi momwe utsogoleri wa boma la Tonse ukuyendetsera dziko lino. Mwa zina, iwo akudzudzula tsankho posankhana maudindo lomwe akuti lamanga nthenje m'dziko muno
Female
katangale yemwe akuti wakhazikika ku nyumba ya boma ndi nthambi zina komanso kukwera mitengo kwa katundu osiyanasiyana kuphatikizapo mafuta ophikira ndi a galimoto
katangale yemwe akuti wakhazikika ku nyumba ya boma ndi nthambi zina komanso kukwera mitengo kwa katundu osiyanasiyana kuphatikizapo mafuta ophikira ndi a galimoto
Female
Apolisi ku Nkhotakota atsekera mchitokosi amuna awiri kaamba kowaganizira kuti athyola nyumba ndi kuba katundu osiyanasiyana pa mudzi wa Ntonya wa m’bomalo
Apolisi ku Nkhotakota atsekera mchitokosi amuna awiri kaamba kowaganizira kuti athyola nyumba ndi kuba katundu osiyanasiyana pa mudzi wa Ntonya wa m’bomalo
Female
Mneneri wa polisi ya Nkhotakota, Paul Malimwe, wati amunawa ndi a Pilirani Zalamatowe komanso a Andrea Piason omwe akuganizilidwa kuti anapalamula mlanduwu mwezi watha
Mneneri wa polisi ya Nkhotakota, Po Malimwe, wati amunawa ndi a Pilirani Zalamatowe komanso a Andileya Piyasoni omwe akuganizilidwa kuti anapalamula mlanduwu mwezi watha
Female
Malimwe wati anthuwa agwidwa Sabata yatha ndipo kuti wina mwa katunduyu yemwe ndi kuphatikizapo wailesi za kanema wapezeka m’boma la Ntchitsi komwe amagulitsidwa
Malimwe wati anthuwa agwidwa Sabata yatha ndipo kuti wina mwa katunduyu yemwe ndi kuphatikizapo wailesi za kanema wapezeka m’boma la Ntchitsi komwe amagulitsidwa
Female
Mneneri wa polisi ya Nkhotakota-yu wati apolisi atengera anthuwa ku bwalo la milandu posachedwapa komwe akayankhe milandu yothyola nyumba komanso kuba katundu
Mneneri wa polisi ya Nkhotakota-yu wati apolisi atengera anthuwa ku bwalo la milandu posachedwapa komwe akayankhe milandu yothyola nyumba komanso kuba katundu
Female
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Saulos Chilima wanyamuka m'dziko muno lero kupita ku Dubai m'dziko la United Arab Emirates (UAE) komwe akaimilire dziko lino
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Saulosi Chilima wanyamuka m'dziko muno lero kupita ku Dubai m'dziko la yunaitedi alabu emiletsi (yueii) komwe akaimilire dziko lino
Female
pa chiontsero cha za malonda chomwe dziko-lo likuchititsa. Malingana ndi kalata yomwe mneneri mu ofesi ya a Chilima, Pilirani Phiri watulutsa
pa chiontsero cha za malonda chomwe dzikolo likuchititsa. Malingana ndi kalata yomwe mneneri mu ofesi ya a Chilima, Pilirani Phiri watulutsa
Female
wachiwiri kwa mtsogoleriyu akukaimilira dziko lino m'malo mwa President Lazarus Chakwera. Kalatayi yati a Chilima akakhala m'dzikoli mpaka pa 21 November chaka chomwe chino
wachiwiri kwa mtsogoleriyu akukaimilira dziko lino m'malo mwa Pulazidenti Lazalasi Chakwera. Kalatayi yati a Chilima akakhala m'dzikoli mpaka pa twente wani Novemba chaka chomwe chino
Female
ndipo akatero azapitilira ku Egypt komwe akakhale nawo pa msonkhano atsogoleri a maiko omwe Ali nawo mu mgwirizano wa malonda wa COMESA
ndipo akatero azapitilira ku ijipiti komwe akakhale nawo pa msonkhano atsogoleri a maiko omwe Ali nawo mu mgwirizano wa malonda wa KOMESA
Female
Maulendo a a Chilima akudza pomwe anthu ena amadzudzula president Chakwera kuti akuchulukitsa maulendo, omwe ena mwa iwo akanatha kutumiza wachiwiri wakeyu kapena nduna ya boma
Maulendo a a Chilima akudza pomwe anthu ena amadzudzula pulezidenti Chakwera kuti akuchulukitsa maulendo, omwe ena mwa iwo akanatha kutumiza wachiwiri wakeyu kapena nduna ya boma
Female
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu ogula katundu osiyana-siyana m’dziko muno la CAMA ladzudzula mabungwe opopa ndi kugulitsa madzi
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu ogula katundu osiyana-siyana m’dziko muno la KAMA ladzudzula mabungwe opopa ndi kugulitsa madzi
Female
kaamba kolephera kutumikira makasitomala awo moyenera, ngakhale mabungwewa amakhala akukweza mitengo ya madzi
kaamba kolephera kutumikira makasitomala awo moyenera, ngakhale mabungwewa amakhala akukweza mitengo ya madzi
Female
Mkulu wa bungwe la CAMA, John Kapito wati ndi zomvetsa Chisoni kuti anthu m’mizinda ndi m’madera a dziko lino akukumanabe ndi zokhoma
Mkulu wa bungwe la KAMA, Joni Kapito wati ndi zomvetsa Chisoni kuti anthu m’mizinda ndi m’madera a dziko lino akukumanabe ndi zokhoma
Female