audio
audioduration (s)
1.12
18.5
raw_text
stringlengths
1
297
normalized_text
stringlengths
1
267
gender
stringclasses
16 values
zomwe m’mboyomu boma kudzera kwa ofalitsa nkhani a Gospel Kazako anatsutsa. Mwambo wa nsembewu uzachitikira ku Ndata komwe ndi ku manda omwe kunayikidwa mtsogoleri wakale wa dziko lino
zomwe m’mboyomu boma kudzera kwa ofalitsa nkhani a Gosipelo Kazako anatsutsa. Mwambo wa nsembewu uzachitikira ku Ndata komwe ndi ku manda omwe kunayikidwa mtsogoleri wakale wa dziko lino
Female
Bingu wa Mutharika, yemwenso anayambitsa gulu la Mulhakho wa Alomwe. Ena mwa alimi ang'ono-ang'ono a m'mudzi mwa mfumu yaikulu Maseya m'boma la Chikwawa
Bingu wa Mutharika, yemwenso anayambitsa gulu la Mulakho wa Alomwe. Ena mwa alimi ang'ono-ang'ono a m'mudzi mwa mfumu yaikulu Maseya m'boma la Chikwawa
Female
auza wachiwiri kwa nduna ya zaulimi, Agnes Mkusankhoma kuti sakugwirizana ndi ganizo la boma loti alandire mbudzi m'malo mwa feteleza mu ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya chaka Chino
auza wachiwiri kwa nduna ya zaulimi, Aginesi Mkusankhoma kuti sakugwirizana ndi ganizo la boma loti alandire mbudzi m'malo mwa feteleza mu ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya chaka Chino
Female
Alimiwa ati boma likanaukira bwino za vuto la njala lomwe lingaze ngati ena mwa iwo saloledwa kuchita ulimi wa mbeu posinthanitsa ndi ulimi wa ziweto
Alimiwa ati boma likanaukira bwino za vuto la njala lomwe lingaze ngati ena mwa iwo saloledwa kuchita ulimi wa mbeu posinthanitsa ndi ulimi wa ziweto
Female
Iwo amayankhula izi pomwe wachiwiri kwa ndunayi inakayendera pa Malo ochitira ulimi a Sande Scheme a m'bomali komwenso kwatumphuka zokhoma zochuluka zomwe alimiwa akukumana nawo
Iwo amayankhula izi pomwe wachiwiri kwa ndunayi inakayendera pa Malo ochitira ulimi a Sande Sikimu a m'bomali komwenso kwatumphuka zokhoma zochuluka zomwe alimiwa akukumana nawo
Female
zomwe ndi monga kusowekera zipangizo za makono zochitira ulimi. Poyankhapo pa nkhani ya ulimi wa ziweto
zomwe ndi monga kusowekera zipangizo za makono zochitira ulimi. Poyankhapo pa nkhani ya ulimi wa ziweto
Female
Mai Mkusankhoma anati anthuwa Ali ndi Ufulu osankha pakati pa feteleza ndi ziweto malingana ndi kusankha kwawo
Mai Mkusankhoma anati anthuwa Ali ndi Ufulu osankha pakati pa feteleza ndi ziweto malingana ndi kusankha kwawo
Female
M'mbuyomu, boma linati alimi 30 thousand a maboma a Nsanje ndi Chikwawa akhala ndi mwai opeza mbuzi imodzi aliyense ndipo azilipira ndalama zokwana 7,500 kwacha
M'mbuyomu, boma linati alimi fete sauzande a maboma a Nsanje ndi Chikwawa akhala ndi mwai opeza mbuzi imodzi aliyense ndipo azilipira ndalama zokwana seveni sauzande faifi handiledi kwacha
Female
monga zizikhalira ndi thumba limodzi la feteleza. Yemwe anakhalapo Wachiwiri kwa sipikala wa nyumba ya Malamulo Clement Chiwaya wazipha poziwombera ndi mfuti
monga zizikhalira ndi thumba limodzi la feteleza. Yemwe anakhalapo Wachiwiri kwa sipikala wa nyumba ya Malamulo kilementi Chiwaya wazipha poziwombera ndi mfuti
Female
mu ofesi ya kalaliki wa Nyumba ya Malamulo a Fiona Kalemba. M'neneri wa Nyumba ya Malamulo a Ian Mwenye atsimikiza nkhaniyi ponena kuti bambo Clement Chiwaya aziwombera ndi mfutiyo
mu ofesi ya kalaliki wa Nyumba ya Malamulo a Fiyona Kalemba. M'neneri wa Nyumba ya Malamulo a Ian Mwenye atsimikiza nkhaniyi ponena kuti bambo kilemenyi Chiwaya aziwombera ndi mfutiyo
Female
m’mawa wa lero la Chinayi mu ofesi ya a Kalemba. Ma repoti akusonyeza kuti a Chiwaya aziwombera kaamba kotopa ndi kuyendera ku nyumba ya malamulo kukafuna za phindu lomwe amayenera kulandira ngati Wachiwiri kwa sipikala opuma
m’mawa wa lero la Chinayi mu ofesi ya a Kalemba. Ma repoti akusonyeza kuti a Chiwaya aziwombera kaamba kotopa ndi kuyendera ku nyumba ya malamulo kukafuna za phindu lomwe amayenera kulandira ngati Wachiwiri kwa sipikala opuma
Female
Pakadali pano thupi la Malemu clement Chiwaya alitengera ku nyumba ya Chisoni ya Kamuzu Central mu mzinda wa Lilongwe
Pakadali pano thupi la Malemu kilementi Chiwaya alitengera ku nyumba ya Chisoni ya Kamuzu sentilo mu mzinda wa Lilongwe
Female
Bwalo lalikulu la milandu ku Blantyre la Chiwiri sabata yamawa likuyembekezeka kuzapereka chilango chake kwa mpondamatiki Thomson Mpinganjira
Bwalo lalikulu la milandu ku Bulantaya la Chiwiri sabata yamawa likuyembekezeka kuzapereka chilango chake kwa mpondamatiki Thomusoni Mpinganjira
Female
yemwe anapezeka olakwa pa mlandu ofuna kupereka ziphuphu kwa Oweruza mlandu. Oweruza mlandu ku bwaloli Dorothy DeGabrielle ndi yemwe akuyembekezeka kudzapereka chilangochi
yemwe anapezeka olakwa pa mlandu ofuna kupereka ziphuphu kwa Oweruza mlandu. Oweruza mlandu ku bwaloli Dolofe DeGabuliela ndi yemwe akuyembekezeka kudzapereka chilangochi
Female
kwa a Mpinganjira omwe pakadali pano akusungidwa ku ndende ya Chichiri mu mzinda wa Blantyre
kwa a Mpinganjira omwe pakadali pano akusungidwa ku ndende ya Chichiri mu mzinda wa bulantaya
Female
A Mpinganjira anapezeka olakwa pa mlandu oti amafuna kupereka ziphuphu kwa Oweruza asanu omwe ankamva mlandu wokhudza chisankho cha Mtsogoleri mchaka cha 2019
A Mpinganjira anapezeka olakwa pa mlandu oti amafuna kupereka ziphuphu kwa Oweruza asanu omwe ankamva mlandu wokhudza chisankho cha Mtsogoleri mchaka cha twente naintini
Female
Sabata yatha akulu-akulu a ndende ya Chichiri anatengera a Mpinganjira ku chipatala cha Kamuzu Central komwe amakawapima pa nthenda yomwe akudwala yokhuza ubongo
Sabata yatha akulu-akulu a ndende ya Chichiri anatengera a Mpinganjira ku chipatala cha Kamuzu sentilo komwe amakawapima pa nthenda yomwe akudwala yokhuza ubongo
Female
Usiku wapitawu, apolisi ku Lilongwe atsekera mchitokosi madalaivala komanso atsogoleri a bungwe la Truck Drivers Association of Malawi omwe pamodzi ndi okwana asanu ndi awiri (7)
Usiku wapitawu, apolisi ku Lilongwe atsekera mchitokosi madalaivala komanso atsogoleri a bungwe la thilaki dilaivazi asosiyeshoni ofu Malawi omwe pamodzi ndi okwana asanu ndi awiri (seveni)
Female
pa zifukwa zomwe apolisiwa sanafotokoze kufikira pano. Poyankhula ndi nyumba ina yofalitsa nkhani m’dziko muno
pa zifukwa zomwe apolisiwa sanafotokoze kufikira pano. Poyankhula ndi nyumba ina yofalitsa nkhani m’dziko muno
Female
mneneri wa bungweli, Paul Kachitsa watsimikiza za izi ndipo wati akuganizira kuti izi ndi chifukwa cha kunyanyala ntchito komwe madalaivalawa akuchita pofuna kukamiza mabwana awo kuti athane ndi zina mwa nkhawa zawo
mneneri wa bungweli, Po Kachitsa watsimikiza za izi ndipo wati akuganizira kuti izi ndi chifukwa cha kunyanyala ntchito komwe madalaivalawa akuchita pofuna kukamiza mabwana awo kuti athane ndi zina mwa nkhawa zawo
Female
Kachitsa watinso bungwe lawo lalandira malipoti oti apolisi amenya mlembi wa bungweli, Mphatso Mollen pomwe anapita kukafufuza za anthu omangidwawa ku polisi ya Kanengo
Kachitsa watinso bungwe lawo lalandira malipoti oti apolisi amenya mlembi wa bungweli, Mphatso Moleni pomwe anapita kukafufuza za anthu omangidwawa ku polisi ya Kanengo
Female
Pakadali pano, mneneri wa apolisi m’dziko muno, James Kadazera wapempha nthawi yokwanira kuti afufuze asanayankhulepo kanthu
Pakadali pano, mneneri wa apolisi m’dziko muno, Jamusi Kadazera wapempha nthawi yokwanira kuti afufuze asanayankhulepo kanthu
Female
Madalaivala a galimoto zikulu-zikulu akunyanyala ntchito ati, mwa zina, pofuna kuti mabwana awo awakwezere malipiro
Madalaivala a galimoto zikulu-zikulu akunyanyala ntchito ati, mwa zina, pofuna kuti mabwana awo awakwezere malipiro
Female
Izi zadzetsa nkhawa yoti zinthu zina zofunikira monga mafuta zitha kuyamba kusowa m’dziko muno ngakhale bungwe loona la mphanvu za m’bweleza, magetsi ndi zina la MERA lati dziko lino liri kale ndi mafuta okwanira
Izi zadzetsa nkhawa yoti zinthu zina zofunikira monga mafuta zitha kuyamba kusowa m’dziko muno ngakhale bungwe loona la mphanvu za m’bweleza, magetsi ndi zina la MERA lati dziko lino liri kale ndi mafuta okwanira
Female
Usiku wapitawu, zinthunzi pa masamba a mchezo zimaonetsa galimoto zikuima pa mizere itali-itali m’malo othilira mafuta ati kaamba koti malo ena mafuta anali atatha kale
Usiku wapitawu, zinthunzi pa masamba a mchezo zimaonetsa galimoto zikuima pa mizere itali-itali m’malo othilira mafuta ati kaamba koti malo ena mafuta anali atatha kale
Female
Mtembo wapezeka mnyumba ina ku Bangwe mu mzinda wa Blantyre ngakhale anthu anali ataika kale thupi la malemuyu
Mtembo wapezeka mnyumba ina ku Bangwe mu mzinda wa bulantaya ngakhale anthu anali ataika kale thupi la malemuyu
Female
Mtolankhani wathu, Gift Maloya yemwe wathamangira ku malo omwe izi zikuchitika wayankhula ndi mfumu Mondiwa ya mdera la mfumu yaikulu Machinjiri
Mtolankhani wathu, Gifiti Maloya yemwe wathamangira ku malo omwe izi zikuchitika wayankhula ndi mfumu Mondiwa ya mdera la mfumu yaikulu Machinjiri
Female
yomwe yati akuganizira kuti mtembowu omwe ndi wa mwana wa mtsikana unaiwalidwa mnyumba pa nthawi yomwe anthu amapita ku manda
yomwe yati akuganizira kuti mtembowu omwe ndi wa mwana wa mtsikana unaiwalidwa mnyumba pa nthawi yomwe anthu amapita ku manda
Female
Mfumuyi yati izi zachitika chifukwa anthu sanatsate mwambo wa bokosi omwe umati siliyenera kukhala lotseka pa nthawi yomwe sanaikemo thupi koma pa nthawiyi, linali lotseka
Mfumuyi yati izi zachitika chifukwa anthu sanatsate mwambo wa bokosi omwe umati siliyenera kukhala lotseka pa nthawi yomwe sanaikemo thupi koma pa nthawiyi, linali lotseka
Female
M'mau ake, mwini mbumba yofeledewayi, a Godfrey Nazombe ati mwanayu anamwalilira ku chipatala kutsatira ngozi ya moto yomwe inamubweretsera mabala ochuluka mpaka kumwalira
M'mau ake, mwini mbumba yofeledewayi, a Godfifule Nazombe ati mwanayu anamwalilira ku chipatala kutsatira ngozi ya moto yomwe inamubweretsera mabala ochuluka mpaka kumwalira
Female
Pakadali pano, thupili aliikanso m'manda ku Bangwe komweko. Anthu omwe abale awo anayikidwa m’manda a pa Desert ku Bangwe mu mzinda wa Blantyre
Pakadali pano, thupili aliikanso m'manda ku Bangwe komweko. Anthu omwe abale awo anayikidwa m’manda a pa Dezeti ku Bangwe mu mzinda wa Bulantaya
Female
ati ndi okhumudwa ndi m’chitidwe wa anthu ena omwe asanduta mandawa ngati malo ochezerapo. Mtolakhani wathu Gift Maloya atayendera mandawa
ati ndi okhumudwa ndi m’chitidwe wa anthu ena omwe asanduta mandawa ngati malo ochezerapo. Mtolakhani wathu Gifiti Maloya atayendera mandawa
Female
anapeza anthu atakhala pa mitumbila komanso ziliza uku akucheza komanso akudya nzimbe, ndipo ena anakhala kumawonera Mpira pa bwalola masewero lomwe liri pafupi ndi mandawo
anapeza anthu atakhala pa mitumbila komanso ziliza uku akucheza komanso akudya nzimbe, ndipo ena anakhala kumawonera Mpira pa bwalola masewero lomwe liri pafupi ndi mandawo
Female
mverani zambiri za nkhaniyi ndi nkhani zina mu nkhani zathu za 7 koloko m'mawa uno
mverani zambiri za nkhaniyi ndi nkhani zina mu nkhani zathu za seveni koloko m'mawa uno
Female
Pali malipoti oti sitima ya ku Mozambique, nambala yake K563 yagunda ndi kupha mkulu wina ochita kabaza wa njinga ya moto pa mudzi wa Kanono m'boma la Neno
Pali malipoti oti sitima ya ku Mozambiki, nambala yake keyi faifi sikisi fili yagunda ndi kupha mkulu wina ochita kabaza wa njinga ya moto pa mudzi wa Kanono m'boma la Neno
Female
Mneneri wa polisi ya Neno, Austin Kamwendo watsimikiza za ngoziyi ponena kuti yachitika m'mawa wa lero.Tikupatsirani zambiri zokhuza nkhaniyi mu nkhani zathu zotsatira
Mneneri wa polisi ya Neno, ositini Kamwendo watsimikiza za ngoziyi ponena kuti yachitika m'mawa wa lero.Tikupatsirani zambiri zokhuza nkhaniyi mu nkhani zathu zotsatira
Female
Boma lapempha anthu kuti akalandire Katemera oteteza ku mliri wa COVID-19 ponena izafika nthawi yomwe katemerayu azizafunika koma samazapezeka okwanira m’dziko muno
Boma lapempha anthu kuti akalandire Katemera oteteza ku mliri wa Kovidi-naintini ponena izafika nthawi yomwe katemerayu azizafunika koma samazapezeka okwanira m’dziko muno
Female
Nduna ya zofalitsa nkhani, Gospel Kazako ndi yomwe yapereka langizoli dzulo pa msonkhano wa atolankhani omwe anachititsa pamodzi ndi akulu-akulu a komiti yapadera ya mtsogoleri wa dziko lino Yolimbana ndi mliriwu
Nduna ya zofalitsa nkhani, Gosipelo Kazako ndi yomwe yapereka langizoli dzulo pa msonkhano wa atolankhani omwe anachititsa pamodzi ndi akulu-akulu a komiti yapadera ya mtsogoleri wa dziko lino Yolimbana ndi mliriwu
Female
Msonkhanowu cholinga chake chinali kufotokozera zomwe komitiyi yakhazikitsa itaunikanso zina mwa ndondomeko zopewera mliriwu
Msonkhanowu cholinga chake chinali kufotokozera zomwe komitiyi yakhazikitsa itaunikanso zina mwa ndondomeko zopewera mliriwu
Female
A Kazako ati dziko lino liri ndi Katemera ochuluka pakadali pano ndipo ndi koyenera kuti anthu akabaitse asanathe mphanvu
A Kazako ati dziko lino liri ndi Katemera ochuluka pakadali pano ndipo ndi koyenera kuti anthu akabaitse asanathe mphanvu
Female
Malingana ndi ndunayi, komitiyi yagwirizana kuti a zaumoyo ayamba kutengera katemerayu m’malo momwe muzisonkhana anthu monga m’mabwalo a masewero
Malingana ndi ndunayi, komitiyi yagwirizana kuti a zaumoyo ayamba kutengera katemerayu m’malo momwe muzisonkhana anthu monga m’mabwalo a masewero
Female
ndi cholinga chofuna kufikira anthu ochuluka ndi Katemera. Iwo adandaulanso kuti anthu sakutsatira ndondomeko zopewera kufala kwa mliriwu ponena kuti izi zikuika pa chiopsezo umoyo wa anthu ochuluka
ndi cholinga chofuna kufikira anthu ochuluka ndi Katemera. Iwo adandaulanso kuti anthu sakutsatira ndondomeko zopewera kufala kwa mliriwu ponena kuti izi zikuika pa chiopsezo umoyo wa anthu ochuluka
Female
Mphunzitsi wina wazaka 27 zakubadwa wapa sukulu ya Pulayimale ya Vikwa m’boma la Kasungu ali m’manja mwa apolisi pomuganizira kuti wapereka pathupi kwa mwana wa Standard 6
Mphunzitsi wina wazaka twente seveni zakubadwa wapa sukulu ya Pulayimale ya Vikwa m’boma la Kasungu ali m’manja mwa apolisi pomuganizira kuti wapereka pathupi kwa mwana wa Sitandade sekisi
Female
Wofalitsa nkhani za apolisi m’chigawo cha pakati, Henry Mnjere, watsimikiza za nkhaniyi pomwe wati mphunzitsiyu zina lake ndi Thokozani Mphangwe
Wofalitsa nkhani za apolisi m’chigawo cha pakati, Henele Mnjere, watsimikiza za nkhaniyi pomwe wati mphunzitsiyu zina lake ndi Thokozani Mphangwe
Female
Malingana ndi Mjere, mphunzitsi-yu ananyengelera mwanayu, yemwe ndi wazaka 16 zakubadwa, kuti amukhozetsa Mayeso akumapeto kwa teremu akagona naye, zomwe mwanayu anavomera mpaka kutenga pathupipo
Malingana ndi Mjere, mphunzitsiyu ananyengelera mwanayu, yemwe ndi wazaka sikisitini zakubadwa, kuti amukhozetsa Mayeso akumapeto kwa teremu akagona naye, zomwe mwanayu anavomera mpaka kutenga pathupipo
Female
Apolisi m’dziko muno amanga apolisi amnzawo okwana awiri komanso anthu ena okwana atatu omwe amagwira ntchito ku nthambi ina ya boma powaganizira kuti akhala akupanga kalata za chinyengo
Apolisi m’dziko muno amanga apolisi amnzawo okwana awiri komanso anthu ena okwana atatu omwe amagwira ntchito ku nthambi ina ya boma powaganizira kuti akhala akupanga kalata za chinyengo
Female
zomwe amazigwiritsa ntchito pokuba ndalama za misonkho. Anthu ochita malonda a kabaza wa njinga za moto m’dziko muno adandaula kaamba ka m’chitidwe wa uchifwamba omwe akukukmana nawo
zomwe amazigwiritsa ntchito pokuba ndalama za misonkho. Anthu ochita malonda a kabaza wa njinga za moto m’dziko muno adandaula kaamba ka m’chitidwe wa uchifwamba omwe akukukmana nawo
Female
Poyankhula ndi Ndirande FM, anthuwa ati ndi okhumudwa kuti anthu ena omwe akumakhala ngati ndi okwera ndi omwe akumawachita chipongwechi
Poyankhula ndi Ndirande efuemu, anthuwa ati ndi okhumudwa kuti anthu ena omwe akumakhala ngati ndi okwera ndi omwe akumawachita chipongwechi
Female
Wa pa mpando wa gulu la anthu ochita kabazayu pa Somanje ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre, Ali Laston wati adindo akuyenera kuchitapo kanthu mwa nsanga pa vutoli
Wa pa mpando wa gulu la anthu ochita kabazayu pa Somanje ku Ndirande mu mzinda wa Bulantaya, Ali Lasitoni wati adindo akuyenera kuchitapo kanthu mwa nsanga pa vutoli
Female
polingalira kuti zinthu zafika povuta. M’modzi mwa anthuwa, Chisomo Harry yemwe amachitanso kabaza ku Ndirande komweko
polingalira kuti zinthu zafika povuta. M’modzi mwa anthuwa, Chisomo Hale yemwe amachitanso kabaza ku Ndirande komweko
Female
wati anthu a upanduwa akumawachitanso chipongwe monga kuwamenya, kuwavulaza ngakhale kupha ena mwa iwo
wati anthu a upanduwa akumawachitanso chipongwe monga kuwamenya, kuwavulaza ngakhale kupha ena mwa iwo
Female
Pamene kumbali yake, Issah Samuel wati mchitidwewu sunakhuze dera la Ndirande lokha koma dziko lonse la Malawi, zomwe zikusonyeza kuti chitetezo sichili bwino m’dziko muno
Pamene kumbali yake, aizeki Samuele wati mchitidwewu sunakhuze dera la Ndirande lokha koma dziko lonse la Malawi, zomwe zikusonyeza kuti chitetezo sichili bwino m’dziko muno
Female
Asilikali a gulu la nkhondo la Malawi Defense Force (MDF) ati mawa lachitatu ayeselera galimoto zomwe a gululi limagwiritsa ntchito kosungitsa bata mu ina mwa misewu ya mu mzinda wa Lilongwe
Asilikali a gulu la nkhondo la Malawi Difensi fosi (emudiefu) ati mawa lachitatu ayeselera galimoto zomwe a gululi limagwiritsa ntchito kosungitsa bata mu ina mwa misewu ya mu mzinda wa Lilongwe
Female
Ogwilizira udindo wa mneneri wa gulu la MDF, Kelvin Mulelemba wati izi zichitika kuyambira nthawi ya 9 koloko m'mawa ndipo walangiza anthu kuti asadzachite mantha alionse poti izangokhala ntchito yoyeselera chabe
Ogwilizira udindo wa mneneri wa gulu la emudiefu, Keovini Mulelemba wati izi zichitika kuyambira nthawi ya naini koloko m'mawa ndipo walangiza anthu kuti asadzachite mantha alionse poti izangokhala ntchito yoyeselera chabe
Female
Malingana ndi kalata yomwe MDF yatulutsa, kuyeselera galimotoku kuzachitika kuyambira ku likulu la nthambiyi ku Kamuzu Baracks kudutsira msewu wa Chidzanja kukathera ku mitundu
Malingana ndi kalata yomwe emudiefu yatulutsa, kuyeselera galimotoku kuzachitika kuyambira ku likulu la nthambiyi ku Kamuzu Balakisi kudutsira msewu wa Chidzanja kukathera ku mitundu
Female
Mtsikana wa zaka 22, Caroline Botha, yemwe anamangidwa kaamba konamiza anthu kuti iye ndi namwino komanso kubera odwala pa chipatala cha Area 25 mu mzinda wa Lilongwe
Mtsikana wa zaka twente thu, kalolini Botha, yemwe anamangidwa kaamba konamiza anthu kuti iye ndi namwino komanso kubera odwala pa chipatala cha eliya twente faifi mu mzinda wa Lilongwe
Female
amulamula kupereka chindaputsa cha ndalama zokwana 90 thousand kwacha. Bambo wina wa zaka 23 zakubadwa, Steven Lucius ali m’chitokosi cha apolisi pomuganizira kuti wapha mkazi wake Dorothy William
amulamula kupereka chindaputsa cha ndalama zokwana nainte sauzande kwacha. Bambo wina wa zaka twente fili zakubadwa, Sitivini lisiyasi ali m’chitokosi cha apolisi pomuganizira kuti wapha mkazi wake Dolofe wiliyamu
Female
atamupeza ali ndi mamuna wina m’nyumba. Bwalo la High Court mu mzinda wa Blantyre lati President Lazarus Chakwera anaphwanya malamulo pobwezeletsa pa mpando Noah Dalasi ngati mfumu yaikulu Ngabu
atamupeza ali ndi mamuna wina m’nyumba. Bwalo la Hayi khoyi mu mzinda wa Bulantaya lati Pulezidentit Lazalasi Chakwera anaphwanya malamulo pobwezeletsa pa mpando Nowa Dalasi ngati mfumu yaikulu Ngabu
Female
Apolisi m’boma Ntchisi ati amanga mphunzitsi wina wa sukulu yapulayimale ya Chitundu, Zuzeni Banda, pa mlandu woti akukhunzidwa ndikufukulidwa kwa manda amunthu wakhungu la achi-albino
Apolisi m’boma Ntchisi ati amanga mphunzitsi wina wa sukulu yapulayimale ya Chitundu, Zuzeni Banda, pa mlandu woti akukhunzidwa ndikufukulidwa kwa manda amunthu wakhungu la achi alubilo
Female
Mneneri wa apolisi m’bomali, Richard Kaponda , wati mphunzitsiyu akumuganizira kuti anapalamula mlanduwu pa 9 Mwezi uno m’dera la mfumu yaikulu Vusojere m’boma lomweli
Mneneri wa apolisi m’bomali, Litchadi Kaponda , wati mphunzitsiyu akumuganizira kuti anapalamula mlanduwu pa naini Mwezi uno m’dera la mfumu yaikulu Vusojere m’boma lomweli
Female
Apolisi ku Dedza akusunga m’chitokosi bambo wa zaka 90 zakubadwa, Lester Dunken, pomuganizira kuti wagwilira azukulu ake awiri azaka zapakati pa 10 ndi 11
Apolisi ku Dedza akusunga m’chitokosi bambo wa zaka nainte zakubadwa, Lesita Dankeni, pomuganizira kuti wagwilira azukulu ake awiri azaka zapakati pa teni ndi leveni
Female
Ofalitsa nkhani pa polisi ya Dedza, Cassim Manda, wati mkulu-yu wamangidwa loweruka lapitali m’mudzi mwa Kafunda mfumu yaikulu Kachere m’bomali
Ofalitsa nkhani pa polisi ya Dedza, kasimu Manda, wati mkuluyu wamangidwa loweruka lapitali m’mudzi mwa Kafunda mfumu yaikulu Kachere m’bomali
Female
Apolisi ku Dedza akusunga m'chitokosi bambo wa zaka 90 zakubadwa, Lester Dunken kaamba komuganizira kuti wagwilira azukulu ake awiri azaka khumi komanso khumi ndi chimodzi
Apolisi ku Dedza akusunga m'chitokosi bambo wa zaka nainte zakubadwa, Lesita Dankeni kaamba komuganizira kuti wagwilira azukulu ake awiri azaka khumi komanso khumi ndi chimodzi
Female
Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi ku polisi ya Dedza, Cassim Manda wati apolisi akuganizira kuti mkuluyu wakhala akupalamula mlanduwu
Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi ku polisi ya Dedza, Kasimu Manda wati apolisi akuganizira kuti mkuluyu wakhala akupalamula mlanduwu
Female
kuyambira chaka chatha koma amawanyengelera kuti asaulule powapasa ndalama yokwana K100 ngati chiseka pa kamwa
kuyambira chaka chatha koma amawanyengelera kuti asaulule powapasa ndalama yokwana wani handed kwacha ngati chiseka pa kamwa
Female
M’modzi mwa akatswiri omenyera ufulu wa anthu komanso katswiri oyankhulapo pa zinthu zosiyanasiyana, Rafiq Hajat wamwalira
M’modzi mwa akatswiri omenyera ufulu wa anthu komanso katswiri oyankhulapo pa zinthu zosiyanasiyana, Rafiki Hajati wamwalira
Female
Malipoti akuti a Hajat amwalira m’mawa wa lero lolemba atadwala nthenda ya mtima
Malipoti akuti a Hajati amwalira m’mawa wa lero lolemba atadwala nthenda ya mtima
Female
Malemuyu analinso mkulu wa bungwe la Institute for Policy Interaction in Malawi. Malingana ndi malipoti a tsamba la pa internet la nyuzipepala ya Nation Publications Limited
Malemuyu analinso mkulu wa bungwe la insichuti fo polise intalakishoni ini Malawi. Malingana ndi malipoti a tsamba la pa intaneti la nyuzipepala ya neshono pabulikeshonzi Limitedi
Female
a kubanja kwa a Hajat ati mkuluyu wamwalira pomwe anali akukonza dongosolo lomutumiza ku chipatala cha ku South Africa komwe amati akalandire thandizo
a kubanja kwa a Hajati ati mkuluyu wamwalira pomwe anali akukonza dongosolo lomutumiza ku chipatala cha ku saufi afilika komwe amati akalandire thandizo
Female
Iwo anabadwa pa 14 September ndipo amwalira ali ndi zaka 55. Pakadali pano, zambiri zokhuza dongosolo loika m’manda thupi la malemu Hajat akuti zilengezedwabe
Iwo anabadwa pa fotini sepitemba ndipo amwalira ali ndi zaka fifite faifi. Pakadali pano, zambiri zokhuza dongosolo loika m’manda thupi la malemu Hajati akuti zilengezedwabe
Female
Mfumu yaikulu Kaduya ya m’boma la Phalombe yalangiza anthu m’dziko muno kuti apewe kumafananiza bungwe la Mulhakho wa Alhomwe
Mfumu yaikulu Kaduya ya m’boma la Phalombe yalangiza anthu m’dziko muno kuti apewe kumafananiza bungwe la Mulakho wa Alomwe
Female
ndi chipani cha Democratic Progressive (DPP) ponena kuti ziwirizi ndi zosiyana kwambiri. Mfumu Kaduya yayankhula izi loweruka lapitali ku likulu la bungwe la Mulhakho wa Lhomwe kwa Chonde m’boma la Mulanje
ndi chipani cha Demokilatiki pulogilesivi (Dipipi) ponena kuti ziwirizi ndi zosiyana kwambiri. Mfumu Kaduya yayankhula izi loweruka lapitali ku likulu la bungwe la Mulakho wa aLomwe kwa Chonde m’boma la Mulanje
Female
komwe amakafotokozera atolankhani za momwe zokonzekera za mwambo wa pa chaka wa bungweli zikuyendera. Mfumuyi yati Mulhakho wa Alhomwe ndi gulu la chikhalidwe osati chipani cha ndale monga umo anthu ena amaganizira
komwe amakafotokozera atolankhani za momwe zokonzekera za mwambo wa pa chaka wa bungweli zikuyendera. Mfumuyi yati Mulakho wa Alomwe ndi gulu la chikhalidwe osati chipani cha ndale monga umo anthu ena amaganizira
Female
M’mau ake, wa pa mpando wa gululi, Leston Mulli anati zokonzekera zonse zokhuza mwambowu zafika ku Mapeto poonjezera kuti mwambo wa chaka chino ukhala osiyana kwambiri ndi wa zaka zonse
M’mau ake, wa pa mpando wa gululi, Lesitoni Muli anati zokonzekera zonse zokhuza mwambowu zafika ku Mapeto poonjezera kuti mwambo wa chaka chino ukhala osiyana kwambiri ndi wa zaka zonse
Female
A Mulli ati ndondomeko zithandiza Kupewa kufala kwa mliri wa COVID-19 zaikidwa kale m’chimake ndipo zidzatsatidwa. Mwambo wa Mulhakho Wa Alhomwe wa chaka chino
A Muli ati ndondomeko zithandiza Kupewa kufala kwa mliri wa Kovidi-naintini zaikidwa kale m’chimake ndipo zidzatsatidwa. Mwambo wa Mulakho Wa Alomwe wa chaka chino
Female
uchitika kuyambira pa 8 mpaka pa 10 October kwa Chonde m’boma la Mulanje. Lawyer wa a Thom Mpinganjira, Tamanda Chokhoto wapempha oweruza Dorothy DeGabrielle kuti aganizire za chilango chofewa
uchitika kuyambira pa eiti mpaka pa teni okutoba kwa Chonde m’boma la Mulanje. Loya wa a Thomu Mpinganjira, Tamanda Chokhoto wapempha oweruza Dolofe DeGabuliele kuti aganizire za chilango chofewa
Female
kwa a Mpinganjira pomwe bwalo lizizawagamula. A Chokhoto mwa zina ati mkuluyu ndi munthu wabwino, uku ndi kupalamula kwake koyamba
kwa a Mpinganjira pomwe bwalo lizizawagamula. A Chokhoto mwa zina ati mkuluyu ndi munthu wabwino, uku ndi kupalamula kwake koyamba
Female
amathandiza timu ya mpira wa miyendo ya Mighty Wanderers, ali ndi zaka 60 komanso anayambitsa bank ya FDH choncho sakuyenera chilango chokhwima
amathandiza timu ya mpira wa miyendo ya maite wandilazi, ali ndi zaka sikisite komanso anayambitsa bank ya efudietchi choncho sakuyenera chilango chokhwima
Female
Koma poyankhula ndi Atolankhani, Reyneck Matemba yemwe amaimira bungwe la ACB pa nkhaniyi anati mfundo za a Chokhoto ndi zosamveka
Koma poyankhula ndi Atolankhani, Reyineki Matemba yemwe amaimira bungwe la esibi pa nkhaniyi anati mfundo za a Chokhoto ndi zosamveka
Female
popereka chitsanzo choti bank ya FDH ili ndi utsogoleri wakewake komanso kuti a Mpinganjira akanayamba alingalira asanapalamule milanduyi
popereka chitsanzo choti bank ya efudietchi ili ndi utsogoleri wakewake komanso kuti a Mpinganjira akanayamba alingalira asanapalamule milanduyi
Female
Oweruza Dorothy DeGabrielle wati azaperekabe chigamulo mtsogolomu. A Matemba anaonjezera kuti milandu yomwe apalamula a Mpinganjira ndi yoyenera kukakhala ku ndende basi
Oweruza Dolofe DeGabuliele wati azaperekabe chigamulo mtsogolomu. A Matemba anaonjezera kuti milandu yomwe apalamula a Mpinganjira ndi yoyenera kukakhala ku ndende basi
Female
A Mpinganjira apezeka olakwa pa milandu iwiri mwa milandu isanu ndi umodzi yomwe bungwe la ACB limawaimba
A Mpinganjira apezeka olakwa pa milandu iwiri mwa milandu isanu ndi umodzi yomwe bungwe la esibi limawaimba
Female
Oweruza Dorothy DeGabrielle wachotsanso bail yomwe bwalo la milandu linawapatsa ndipo akuti akawatsekere ku ndende ya Chichiri kufikira azapatsidwe chigamulo
Oweruza Dolofe DeGabuliele wachotsanso belo yomwe bwalo la milandu linawapatsa ndipo akuti akawatsekere ku ndende ya Chichiri kufikira azapatsidwe chigamulo
Female
Oweruza Dorothy DeGabrielle wati umboni wa milandu yomwe a Mpinganjira akuyankha uli mmanja mwa osuma lomwe ndi bungwe la ACB kutsimikizira kuti mkuluyu anachitadi upo ofuna kupereka ziphuphu
Oweruza Dolofe DeGabuliele wati umboni wa milandu yomwe a Mpinganjira akuyankha uli mmanja mwa osuma lomwe ndi bungwe la esibi kutsimikizira kuti mkuluyu anachitadi upo ofuna kupereka ziphuphu
Female
Izi ndi malingana ndi kalata zozukuta umboni zomwe pakadali pano akuwerenga. Iye watinso bwalo liunguza ngati mkuluyu anali ndi upo chabe
Izi ndi malingana ndi kalata zozukuta umboni zomwe pakadali pano akuwerenga. Iye watinso bwalo liunguza ngati mkuluyu anali ndi upo chabe
Female
ofuna kupereka ziphuphu kapena anayesera kupereka ziphuphu kwa ma judge wa molingana ndi umboni
ofuna kupereka ziphuphu kapena anayesera kupereka ziphuphu kwa ma jaji wa molingana ndi umboni
Female
Chitetezo chakhwimitsidwa ku bwalo lalikulu la milandu mu mzinda wa Blantyre pomwe lero bwalolo lipereke chigamulo chake pa nkhani yokhuza upo ofuna kupereka ziphuphu kwa ma judge
Chitetezo chakhwimitsidwa ku bwalo lalikulu la milandu mu mzinda wa Bulantaya pomwe lero bwalolo lipereke chigamulo chake pa nkhani yokhuza upo ofuna kupereka ziphuphu kwa ma jaja
Female
omwe amanva mlandu wa chisankho cha mtsogoleri cha mu 2019 omwe mpondamatiki Thom Mpinganjira amayankha
omwe amanva mlandu wa chisankho cha mtsogoleri cha mutwente naintini omwe mpondamatiki Thomu Mpinganjira amayankha
Female
Kunja kwa bwalolo kulinso gulu la anthu ena omwe akuimba nyimbo komanso kuvina ati kusonyeza umodzi ndi a Mpinganjira
Kunja kwa bwalolo kulinso gulu la anthu ena omwe akuimba nyimbo komanso kuvina ati kusonyeza umodzi ndi a Mpinganjira
Female
Anthu ochuluka pa masamba a mchezo aonetsa kudabwa komanso kugwidwa ndi phwete ndi kanema wina yemwe akuonetsa achitetezo awiri a mtsogoleri wa dziko lino
Anthu ochuluka pa masamba a mchezo aonetsa kudabwa komanso kugwidwa ndi phwete ndi kanema wina yemwe akuonetsa achitetezo awiri a mtsogoleri wa dziko lino
Female
Lazarus Chakwera atanyamula zimkuza mau pa nthawi yomwe a Chakwera amayankhula kwa anthu pa ulendo wawo opita ku Mangochi
Lazalasi Chakwera atanyamula zimkuza mau pa nthawi yomwe a Chakwera amayankhula kwa anthu pa ulendo wawo opita ku Mangochi
Female
Okuba aba zipangizo zomwe ophunzira amayembekezeka kugwiritsa ntchito polembera mayeso a Standard 8 pa sukulu ya Pulayimale ya Chikwawa m’boma la Rumphi
Okuba aba zipangizo zomwe ophunzira amayembekezeka kugwiritsa ntchito polembera mayeso a sitandade eiti pa sukulu ya Pulayimale ya Chikwawa m’boma la Rumphi
Female
Wofalitsa nkhani za apolisi m’chigawo cha ku Mpoto, Maurice Chapola, watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti okubawa aba zipangizozi m’mawa wa lero la Chitatu
Wofalitsa nkhani za apolisi m’chigawo cha ku Mpoto, Molisi Chapola, watsimikiza za nkhaniyi ponena kuti okubawa aba zipangizozi m’mawa wa lero la Chitatu
Female
Koma Mneneri wa a polisiyu, Chapola wati mapepala a mayeso sanabedwe nawo. Pakadali, pano ophunzira pa sukulupa ayamba Kulemba mayeso awo
Koma Mneneri wa a polisiyu, Chapola wati mapepala a mayeso sanabedwe nawo. Pakadali, pano ophunzira pa sukulupa ayamba Kulemba mayeso awo
Female
Ophunzira opitilira 281,000 ndi omwe akuyembekezereka kulemba nawo mayeso a MANEB a standard 8 omwe ayamba lero la Chitatu
Ophunzira opitilira thu handiledi andi eite wani sauzande ndi omwe akuyembekezereka kulemba nawo mayeso a Manebu a sitandade eiti omwe ayamba lero la Chitatu
Female
Ophunzira opitilira 281,000 ndi omwe akuyembekezereka kulemba nawo mayeso a MANEB a standard 8 omwe ayamba lero la Chitatu
Ophunzira opitilira thu handede and eite wani sauzande ndi omwe akuyembekezereka kulemba nawo mayeso a Manebu a sitandade eiti omwe ayamba lero la Chitatu
Female
Izitu zaululika pa msonkhano wa atolankhani omwe unduna wa zamaphunziro pamodzi ndi bungwe lolembetsa mayeso la MANEB
Izitu zaululika pa msonkhano wa atolankhani omwe unduna wa zamaphunziro pamodzi ndi bungwe lolembetsa mayeso la Manebu
Female
komanso nthambi ya asilikali a gulu la nkhondo ya MDF anachititsa la Chiwiri. Malingana ndi bungwe la MANEB
komanso nthambi ya asilikali a gulu la nkhondo ya emudiefu anachititsa la Chiwiri. Malingana ndi bungwe la Manebu
Female
chiwerengerochi ndi chotsika poyerekeza ndi ophunzira omwe analemba mayeso a ngati omwewa chaka chatha chomwe chinali chopitilira 331,000
chiwerengerochi ndi chotsika poyerekeza ndi ophunzira omwe analemba mayeso a ngati omwewa chaka chatha chomwe chinali chopitilira fila handed andi eite wani sauzande
Female
Bungwe lothana ndi ziphuphu komanso Katangale la ACB lakana kufufuza ngati panali za chinyengo pa momwe ntchito yolemba mkulu wa bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (Mera) inayendera
Bungwe lothana ndi ziphuphu komanso Katangale la esibi lakana kufufuza ngati panali za chinyengo pa momwe ntchito yolemba mkulu wa bungwe la Malawi eneje legyuletale ofolite (Mera) inayendera
Female